The Lilongwe high court is today expected to hear the cashgate case for former Malawi Defense Force (MDF) Commander Henry Odillo who is suspected to have swindled K5 billion.
Odillo and five other suspects are to answer charge of misappropriating public money from 2012 up to 2013 during the reign of self-exiled Malawi leader Joyce Banda.
Confirming to the local press, Judiciary spokesperson Mlenga Mvula said the court is set to take the case for proceeding from Friday in Lilongwe.
“Friday has been set for plea and pronouncement of case directions starting from 11 am”. Said Mvula.
He added that one suspect Alexander Banda, is to be tried from South Africa upon completion of the legal process on the matter.
Odillo is among public officers who are reported to have defrauded Malawi government on dubious transactions.
Ine monga olira misonkho yanga misozi imangotsikila m’mimba, chifukwa anthu yawa zawo ndizimodzi amangotiphimba maso basi.
Want to buy a car from BE FORWARD JAPAN? Very simple and easy as you will enjoy a special discount when you use BFS ID REFERRAL NUMBER 294667
STEPS
1] Go to http://www.beforward.jp
2] You will access a range of cars from as low as US $500, browse the cars on the stock and select your car of your choice
3] Click on the car of your choice ,view the pictures ,engine type etc, if you are satisified with it scroll down to the bottom of the page and fill out the fields
4] After you fill out the fields above ,you will receive a quotation from BE FORWARD indicating the amount for the purchase of the car, when you are satisfied with the details ,fill the form and the BFS ID referral number 294667 to enjoy a special discount!
5] Deposit your money in the bank in US$ and transfer it to the BE FORWARD account in Japan. It will take three days to reflect that it has been sent.
6] You are done ! Wait for your car at the port you have chosen at the of two or three months!
Purchase your car today with BE FORWARD and enjoy a special discount when you use BFS ID 296447
Ndi au silu. Chi vampire cheni cheni chija chamu vampire diaries. Fayabon wu bomboclat … fayabon canomind
kupakula mpaka 5bilion eeeeee koma pa Nyasalande kuba kwambiri
Koma big mudayaluratu ndalama za Jet kulikita two pple inu ndi ma stern
igomusiani wina aliyense akasiya udindo wake kapena aka2la pansi undindo mumalimbana naye kut waba ndalama ndi ndani angakhale pamenepo osamuimba mulandu pot aliyense ndi wakuba
Zawathela bwanji a Odilo?,
Fufuzan Kae Kt Wapezeka Olakwa Thn Kuma Comenta Bwio Becareful Mungapeze Nazo Vuto
Zomwe zachitika ku America ndi zomwe zikufunikanso pa Malawi,tidzavotere china chipani osati iwo omwe ali kale m’boma,chifukwa tikapitiliza omwewa adzibabe ndalamazo and maumboni nkumaotcha,dziko li tikawasekerera lidzafika povuta mpaka wanthu nkumaphana kulimbilana zinthu,change is wat we need right now,Wake Up my Malawi.
Inu osaba sadzapezeka kumangovomekeza bas
Confrict of interest brings change. We are the change.
Eeeh koma ada amenewa anamanga nyumba yokwiya kwambili yokhalamo eeeh big up cash gate master munatiyeletsadi m’maso. Anyway but judgement is coming
Should be arrested!
ok?
Aaaaa DPP in court kumwamba mupha anthu kumudzi & 2,000 mukufuna ituluke muona ngati ndinu anzeru
Shaaa!! Zavuta kumpando
Kkkkkkk naye ananyemako kodi kkkkkkk
mwatani anganga nkhaza kuipa nkhope ndi mtima. ma bilion mwadyawo ndi anthu osauka.
Ai koma zinazi iiiiii ce Odillo munawonjeza simpaka kudyetsa kamudzi kanu konse
The government must give him a lesson b4 week
A li ndi mwayi poti achair ali kutali ndi umfumu warerowu adakasowa
They just deserve to be killed …. Rubish
Inuyo muli ndi mphamvu zopha munthu?
Are you interested in the world of FAME??
Getting rich. powerful and famous?
JOINING THE ILLUMINATI BRINGS YOU INTO THE LIMELIGHT
OF
THE WORLD IN
WHICH YOU LIVE IN TODAY. YOUR FINANCIAL DIFFICULTIES
ARE BROUGHT TO AN
END. WE SUPPORT YOU BOTH FINANCIALLY AND
MATERIALLY
TO ENSURE YOU LIVE
A COMFORTABLE LIFE. IT DOES NOT MATTER WHICH PART
OF
THE WORLD YOU
LIVE IN. FROM THE UNITED STATES DOWN TO THE MOST
REMOTE PART OF THE
EARTH, WE BRING YOU ALL YOU WANT. BEING AN
ILLITERATE
OR A LITERATE IS
NOT A BARRIER TO BEING A MILLIONAIRE BETWEEN TODAY
AND THE NEXT TWO
WEEKS. YOU BEING IN THIS OUR OFFICIAL PAGE TODAY
SIGNIFIES THAT IT WAS
ORDERED AND ARRANGED BY THE GREAT LUCIFER THAT
FROM
NOW ON, YOU ARE
ABOUT TO BE THAT REAL AND INDEPENDENT HUMAN YOU
HAVE ALWAYS WISHED YOU
WERE .SO IF YOU ARE INTERESTED IN BECOMING A
MEMBER,
GET BACK TO ME
IMMEDIATELY.. IF YOU JUST WANT TO JOKE, DON’T SEND
ME A
MESSAGE.
REMEMBER THIS, IF YOU CAN ACCEPT THE FIRST STEP, I
ASSURE
YOU, YOU
WILL BE WHAT YOU HAVE EVER WISHED FOR. THANKS.!!!!!! CONTACT US IMMEDIATELY Via Email: [email protected] or [email protected]
kkkk odilo bwanjinso aululu mama kuti ndalama yogulira zida za MDF anadya
5 billion and leaving behind MDF in TATAs not good, we would have too much greed once in power amalawife. Nde akapezeka wolakwa timutani muntguyu timumanga kapena timuuza kuti abwenze makopala athuwa?
eeeeeehhh kwaterera
Next president Henry Odilo
kumagomanga anthu owerengeka pomwe akuba ndichimkwanyanya cha anthu
Ndalamazo mukaba mumadya nokhanokha zikavuta mumamangana nokhanokha boma lokuba zimanganani nde bwino
Eeeeeee koma cashgate anthu ambiri asendeka nayo maka ndi ma comander omwe akukhuzidwa shaaaaaa
kodi nanga maina ena amamveka aja kuti a ACB analandila a anthu omwe akugwila ntchito pano m’boma,kodi maina amenewa atuluka liti? nanga ndichifukwa chani zikuoneka kuti sizikutheka? ndiye kuti cash get yo ikupitilirabe mpaka pano? Mwina titelo kuti khoswe akakhala pa m’khate sapheka? Nanga dziko la britain lati silokomzeka kupeleka thandizo ku dziko la malawi chifukwa chani? Izi ndizimene zikuonetsa kuti this current government is not serious to fight against corruption,but also being involved in this immoral practise,with this malawi will remain the same,corruption reaching it’s climax and it has started bearing fruits which are sour now.
corruption in our country deals only to those pple who were in opposition side,if u steal more kwacha but ur in gvnt side ameneyo akut siwakuba just leave him.
Okey,sir u r right but is this gud?
To be adjourned mumva
Mwinaso samangidwa
Ndichisoni chomwe mulibe mukamaba anthu tikuvutika koma in ndikumanjoya ndidziko lakelomweli, Tayimani muwona!
Kuli Ngat Kutuma Mbava Kti Ikagwre Mbava Inzake Mwachziwikre Nayonso Ikayamba Yapisa Nthumba La Inzakeyo Then Ibwelese Zonyenyeka Kwnako Isunge Onsewa Ndiakuba Bas Kulibe Ndalama Zonse Znathela Mwakachelemu Ndi Ma Hule
He must tell more we need all of them nothing hidden in der world
Dziko lapansi munthu opanda chifundo ndiyemwe akusangalala
Where are others?
komatu 577Bln imandikwanaso bwanji tiyen nazoni
No Jesus No Life
zinapita zinatha or mulimbane naxo palibe phindu or kubweza
Nde unaiyamba2 bwino nkhaniyi,ndimayetsa ukuti wamwalira,anthu oipa ngati amenewa sakuenera kumakhala ndi moyo mpakana lero.
Akagwire ndende basi atibera kwakwana apite basi asaone nkhope
Na dziko la malawi wanthu ndiye walibeladitu. mpaka pano akulibelabe. zovuta kwambili.
Tchifukwa-chake-malawi-tizingokharira-kupempha-vuto-dziko-la-malawi-wina-aliyense-amafuna-kulibera-dzikoli-ndalama-ngati-zimenezi-bwenzi-mutamangira-ma-school-mwina-tithakupuna-kuphunzira-pansi-pamtengo-tithakarira-duka-lanjerwa
Mfiti za anthu,akafele kundende basi
Yooo its alots of money koma pa ndalama zonsenzi anapangapo chani? umva palibe zimangothera achina Patricia Kaliati
Che Mkasa Nde Anaimba Zalamulo!Nati ! lamulo siliwona olemela kapena Osauka!liyenela kugwila Ntchito basi.
Eeee eeeee ndalama zonsezi
Kkkkk koma a James one nkadagula petrol
kkkkkk koma ndemkwiyot mpaka 5litres ya petro?
Iiii zanu izo mxiiiiie
lamuro ligwile ntchito mosayang’ana mbali kapena nkhope dziko lilipamavuto chifukwa cha anthu ngat amenewa.
koma ndikanakhala ine mulandu wokuba mazira mukanandiotcha mxiiiiiiiiiiiii Zanu izo
kkkkkk akanangot no discution wabawekha usalire ena akut timuotche.
aaaaaaaaa Dziko ili zinazi tizingoyang’ana palibe chomwe tingapanga Osauka tilibe mawu? tilinawo koma sangamveke
kkkkkk zimenezo ndizija anaimba Billy zija osauka alibe mau alibe O alibe mau alinawo.
Muva pompano kuti zilibe umboni koma zomwezo achite wina opanda dzina ndi ndalama mayooo ineeeeeeeeee!
Kuti Mulandu Umeneu Uzathe Ine Ntayamba Imvi Mumva Zoti Auimika Pakufunika Mboni Kkkk
Kodi alipo squad eti