Wanderers, Bullets to open Bingu National Stadium

Advertisement
Bingu National Stadium

Old football rivals, Be Forward Wanderers and Nyasa Big Bullets will open the world class Bingu National Stadium in Lilongwe, Malawi24 has the latest information.

The two Blantyre giants meet in the Luso TV bus Ipite Football Fiesta on 2nd January 2017.

Bingu National stadium
Bingu National stadium will host Bullets and Wanderers in two months time.

This development comes barely a few months after government through the Ministry of sports and Culture said the stadium will be ready for use before the end of this year.

Malawi24 understands that the facility will be opened next year. This is surely after 2nd January when the match between Bullets and Nomads will take place.

The 40,000 capacity stadium was expected to be opened in October this year but the Minister responsible Henry Mussa in October said the stadium needed more money so that the stadium should be completed.

According to Mussa the stadium needed over K600 million which was luckily sourced by his ministry for the completion of the magnificent stadium.

The minister said the stadium was remaining with floodlights and the sewer system among others.

Nomads vs Bullets
Bullats and Nomads will meet at the new facility in January.

The wait for the opening of the newly constructed stadium in Lilongwe is now over as the Football Association in collaboration with Luso Tv have set the 2nd of January, 2017 to be the date that the stadium will host a match between Wanderers and Bullets in the Luso TV Bus Ipite football fiesta.

It is with no doubt that Bullets and Wanderers are going to renew their rivalry as the two will be battling it out in a two leg Luso TV bonanza and the winner will go away with a Nissan Civilian 26 seater.

The first match will be played on the 26th of December on Boxing Day whereas the second leg will be played at the Bingu National stadium in Lilongwe on 2nd January, 2017.

The Blantyre football giants match will be the first match that will be hosted at the Bingu National Stadium as the Malawi National Football team has no any international match this year as the team is not participating in any competition and the Malawi FA has not set any friendly game for the team this year.

The Chinese government pumped in 26.6 billion kwacha into the 40,000 capacity stadium project.

Advertisement

222 Comments

 1. i ve just listern to de speech of eric ling’ang’a he said and i quote..stadium wil be opened on 10 decembr,on dis day malawi vs china will open de stadiun..refer zodiak

 2. A FAM penapake kapangani zinthu zoti mutukule mpira osati kulowetsa pansi masewera chomwe chakusangalatsani kuma team wa ndi chiyani kodi simungayatane yakunja na tional team kuti adzamenye FLAMES Kuti mudza mpatse mpata coach amene akuyembekayo ganizani

 3. Today live from Zodiak and analengeza kuti pa 5 December akutsegulira bwalo limeneri and will be Malawi vs China not zomwe munenazi ayi

 4. why not flames to open , why clubs nde tinene kuti flames ikuwopa ku sewera ndi ma team

 5. Nanunso akumipando inu tazikhalani ndi nzeru simungaitane ma neighbers country kuzasangalasako anthu inu koma dyela basi.

 6. Malawi sazatheka kukondera ndi ku mpira komwe ngakhale ineyo ndili wa wanderers chonde ku Malawi kuno matimu aliko ambiri koma eee…. noma/nyas, noma/nyasa. noma/nyasa ee.. koma ziliko nchifukwa chake mpira sukupita patsogolo. Komanso tili ndi tsoka ma president timasankha ife ku Malawi siokonda mpira choncho mbuzi zoyang’anira mpira zimabweretsa zigani zofoyira. Tapezani team ya kunja ie China, Zambia, Zimbabwe, Egypt, etc …. anzathu pa Zambia pompa anayitana GABON potsegulira HERO’S Stadium ku Lusaka. Boma lisaope kuononga ndarama bola tiwonongera zamphindu kuposa cashgate. Koma za noma ndi bullets izo ayi …. tawonera mokwanira madunju

 7. Y only Blantyre teams? Ku lilongwe kulibe mateam? Bwanji osatenga imodzi from bt and the other one from lilongwe kapena mzuzu? Ku fam kwa dzaza ndi anthu anyaupee ndi2

 8. a Malawi, mukulimbikira kut bola stadium ikanaseguliridwa ndi Flames, kodi mkufuna stadium ya sopano izasegulidwe ndi lose?

 9. NEBA LELO TSI MAWA.MPILA WA PAMWA UDAPITA MPILA UMAKHALA NGALAUNDI.MPAKA KUT NYELELE NDI MABOLELA A NYASA.NDAZIWA NDIDAIWALA KUT MASAPOTA NYASA ACHULUKA MBAV,ACHAMA MITU YAWO IDAFA NDI KACHASO WA MUNDILANDEMU.OSAMATHA MAU .

 10. inu zoona bullets mukuipatsa noma?ifetu a bullets tikati derby ndekuti tikumenya ndi tigers nde bwanj simunatipatse ma tiga?

 11. koma ma black out ake amenewa ndee mpila wautsiku uzikhalapo? hahahahaa ine wa bullets koma apa sanasakhe bwino stadium ndi ya national bwedzi itasekulira ndi national team coz apa zikhala ngat mwakondela mbali imodzi coz ma teams asakhidwa apawa ndiochokela BT tiziti ku LL kulibe ma teams oti angasekulire nawo stadium or mukanatenga yaku LL vs BT

 12. Tatopa ndi maganizo oti BULLETS ndi WANDERERS adzasegulire bwalo la Bingu national stadium.Ine ndili wa Bullets koma pankhaniyi sindikugwirizana nazo ngat ndichoncho kulibwino kuyitana mayiko akunja azatiphunzitse mpira. Am not happy at all wth the government decision. AMalawi sitingapambane mpira chifukwa timakonda kuchita zinthu zachangu m’malo mokonza zinthu ife timaonongelathu.

 13. NOMA VS NDUDU FC.China osatopa yasala inanso ku Blantyre kuno ife chomwe timadziwa ndi kupempha ndi kuba(cashgate) basi.

 14. Thumbs up Nyamilandu…….tikayinyenye bullets pa bwalo latsopano. Go komko phiri.

 15. Pezani team yakunja idzasewele ndi team ya Malawi,ndi misonkho ya a Malawi imene ija aliyense asangalale chifukwa zimezi ma club ena adandaula.

 16. Ndikungozimvera chison ,inu kusegulira stadium simungaitanise team from another country lyk south Africa Zambia,Zimbabwe,kaya china yomwe yo nkuzamenya ndi flames ,dzikutanthauza chan kutenga ma club onse akuno Ku BT kut apalane mamba wandikwiisa iwe Malawi na pokhapa apa,

 17. FAM alakwisa kumawanvelako chisoni makochi a Noma akaluzatu amawachosa ntchito sono izi zomwe apanga a FAM sizabwino iyayi

 18. sindinaone ngati yafika pokongola choncho. Maka n’seuo komaso ndikuona ngati udzu m’mbali mwakemo. Pamene Stadium- m’mene ndinaionela ine kunja kulibe n’seu omwe ukuonekao mwaina mwangotitumizila yadziko lina osati Malawi ayi

 19. Bullets ndi Noma are just ordinally teams like Kabwafu football team in Mpherembe Mzimba. Matama thooo!!! akati amenya international football ndiyekut anapita ku Maputo kukamenya ndi Matchangane apo ayi ndiyekut akati ayenda mtunda wautali ndiyekuti anali pa Mzuzu stadium kukamenya ndi Karonga United mapazi anuuuu.

 20. Danken micky musanamize anthu ai,chipatala chachikulu mumzinda wa Pretoria capital city dzina lake ndi steve biko academic hospital ,solomon mahlangu drive msewu wawukulu kumawa kwa pretoria onsewa ndimaina aanthu omwe anathandiza pankhan zawufulu ndie nanga kumalawi kuika dzina lot kamuzu stadium palakwika ndie kt asogoleri ake ndiwofun kutchuka?

 21. Bwanji asankha ma team aku blantryre okha? silver iliko komatso moyale bwanji akanangotengapo imozi if not bwanji akanangoitana national team yadziko lina isewere ndi malawi zachamba eti

 22. Nkhaniyi ndi yabodza ndipo boma silinabwere poyera kuti stadium itsegulidwa tsiku lanji izi tikumva apazi ndi za mmaluwa za a Malawi 24 tisaiwale kuti page imeneyi mbuyomu idabwera ndi nkhani yoti Peter Muthalika wamwalira

 23. Manoma ulalata mpila mpaground man mgati kuli timu yayikulu nde Bullets inuso mumadziwa, pliz cloz your mouth. palibe chisangalalo ngati palibe maule Bullets ndicikoka malawi yose NBB ndi kawawa!!!

 24. Which is which..Some quarters are saying the Stadium will be graced by a match between Malawi nation team against China nation team, and you are saying to the contrary. Hope one of you is saying the truth, but dont know who he is…We are only keeping our fingers crossed till the day of the official opening….

 25. Every one has his/her ups and downs.what matters is percentage of ups should more than downs,for me the late bingu was a great man,the naming of stadium is good

 26. Poti ndibodza komaso ife a central region sitingalore kena kachoke uko kali mamina pa mphuno kuti ndukatsegulira stadium yaku Lilongwe.

  1. Kaya ufune kaya usafune koma udzaona zitachitika who are you kuti uzinena zopusazi apa noma ndi bullets ndi mateam akunja kupepera kapena umbuli eti?

  2. Kwina kulikonse amatenga matimu akulu akulu example southafrica imatenga chiefs ndi pirates kwathuko matimu akulu ndi amenewo usachuluke mzeru iwe

 27. Big up a FAM for your wise decision coz Flames ikanazaluzanso pa bwalo la new one ngati limeneli.
  Poopa kukhumudwisa ambiri mwachita bwino kutenga team yomwe ili ndi ma supporter ankhaninkhani kuposa Flames komanso team imene ili ndi zikho kuposa Flames-yo #BULLETS kuti ikomane ndi team yobadwa kumayambililo #Wanderers angakhale Nebayu za league zimamuvitavuta kkkkkkkkkkkkkkk.
  Koma ndikadakonda Wanderers ikanapanga alliance ndi Nyau fc vs BULLETS kuti zizakome coz apa zotsatila anthu azinziwa kaletu.Wanderers ndi mabwila a BULLETS kkkkkkkkkk.

  1. Tidatuluka chifukwa Eagles idatipepha kuti ikufunisitsa kuti nayonso itengeko cup.Ndiye ife ndioti tili ndi cup kale komnso titenga league tinachiona chabzeru kuwasiila kkkkkkkkkkkkkkk

  2. Ukudwalikadi iweyo Alick standard bank cup siyinafikekutha osayilawako ? Nanganso bwanji muli pa 3 pomada mukapenzeka pa 4 chifukwa chiyani mutamenyanso magame ochuluka ?

  3. A bullets ambiri ndi odwala include iweyo Alick,, si wanderes yomwe inakuonesani msana wa njira koma ndi Blessings Tembo mothandizana ndi Nthuso pipe mikango zinyama zoopsa kkkkkl

  4. Koma iweyo matenda ako ndiowopsya kwambiri moti kupita nawo kuchipatala anthu akakupatsa mpata kuti uwonane ndi doctor mwachangu kkkkkkkkkkkkk.
   BULLETS 43 cups
   Noma 25 cups
   Silver 15 cups
   Wanderers nayo ma cup ena akhala akutha osatenga BULLETS siyoyamba koma sikuti munatisa kumbali ya ma cup.
   Za league ukunziwanso wekha kuti BULLETS itenganso kachitatu mosogozana inu mukutha 15 yrs osatenga kkkkkmkkkkkk

  5. Kodi wakapado fc akuti chani apa wayambapotu matenda ako aja osagwilikawa tinakukunthani pa KB stadium ndiye mukufunaso chani apa iyotu ndi Bingu stadium musaiwale timanyenyanyenya muzabwele mutazola mafuta anu ajatu kkkkkkkkkkkk

  6. Inu abullets pakamwa bwanji?jez yeniyeniyi mmachita kusungunula paint ndikumalembera ma # ndi maina pamsana.mvula itabwera kunapezeka kt jez ya fisha itafufutidwa kunasala ndowe mmalo mwa Kondowe….team iyi ndiyo nyenyeka heavy,,,pa change (half tym)amangofinyirana timadzi ta mmajumbo kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk!!!

 28. Kodi kuchita kuti international stadium eish komadi zikubwera mochedwa Malawi @52years.komaso dzina loti Bingu lo mwaganiza bwanji?

 29. Timvelane osamangotokota apa bullets simagawa kamba bullets ndi noma ikakumana kumakhala ndalama zankhani nkhani nchifukwa chake asankha matimuwa

 30. Chimene chikufunika ndi kukamenya mpira ngati uja amamenya a silver umodzi umodzi osati mukayambe yanu ya phuphuphu ija ndiyetu ndi bwalo limene lija sizikagwilizana

 31. Anthunu mukumago commter ndizonama zomweeti ndakuwuonani imeneyi ndi Malawi24 guyz mawa muiiva ikukaba zina kkkkkkk.

 32. Kumalawi kumandidabwitsa. Maka maka ma presdent ake. Sangapange chitukuko. Osaika maina awo. Things like. Bakili bullets. Bingu high way. Muthalika stadium. Joyce Banda school. Kamudzu stadium. Komatu ndee maiko. Anzathuwa sinanve olo akuti. Mugabe hospital. Zuma stadium. Even Obama white house. Ayi koma kumalawi kokha basi. Dyela nd kufuna kuchukha basi.

  1. Sam nujoma stadium, Namibia. Moi stadium -kenya . Keneth kaunda Airport- Levie mwanawasa stadium-zambia. Olushgan hospital -nigeria . Kagame hospital -rwanda e t c. Muzifufuza kaye za maiko ena , osamangonyoza chilichonse cha ku Malawi. Thats not good man.

  2. Iwe nd ine waenda kwambili ndani?? Chomwe simukundinvetsetsa. Chakuti each fucking presdent. He or she akumaika maina. Pomwe maiko omwe mwanenawo. Mwina nd modzi yekha anapanga. Now lets prove a point. Wina ndani ku zambia nd nigeria.kenya kaya kuti kupatula omwe mwachulawa??? Give me some more. U stil in darkness.

  3. Tichezere ndi nkhani yake yomweyi? alipo ambiri man ndipo zilipo zambiri zatchulidwa mmayina ama president ammayikomo . Ine ndangopereka exampl si nanga mumati nkumalawi konkuno zikuchitika. Mukafuna kuti tibwere ndi list yonse mukhumudwa ndithu

  4. Aaa ndimaziwa. Kuti muyakha chonchi. Man but ine ndayakhulazi. Ndizoona wether u like it or not. Sindikunyoza ziko langa. Koma i am making a point baba.

  5. Danken your right: dzanyanya, umbuli wa anthu ophuzira ndi umenewo chilchonse chimene apanga amafuna aike dzina lawo nde akati azipanga zitukuko ndi ndalama zammatumba mwawo. koma China watithandiza nde mmalomopeleka dzina la ma china nde akuti Bingu for what?

  6. Goodson, Kabichi, mwamuona Damiano. Wasuta cha kukotakota. Koma alibe vuto ndangonva kuti. Watuluka zulo ku chipatala chachikulu ku zomba. Lol

  7. Ku Malawi mpan’gono maiko ena zanyanya,mwachitsanzo ;moses mabhida stadium,lukes moripe stadium,nelson mandela bay stadium,OR Tambo airport jst 2 mentin a few bro kkkkkk!

  8. Hahahaha usandiseketse. Moses mabhida lukas moripe. Or tambo. Nd maina ama presdent aku south africa?? Anakuuza ndani. If this is dream plz someone wake me up. Kkkkk

  9. Maina a wannthu a ndale,nde zikusiyana pati ndi Bingu kungoti u’ve a negative attitude ndi Bingu

  10. No. Ndee sukanati andale. I said presdent. What so hard for u. To undastand what i am saying. Nd ineyo ndikanakhala kuti ndili nd vuto nd bingu. Ndee ndikanena athu onsewo?? I tel u what i give my opinion. Take it or move on nigga

  11. Madala mwanama2 kuno msewu uli onse uli ndidzina la munthu yemwe adatchuka muderalo, Kuli Robert Subukwe Dr, Van Rebeck Dr, Groote Schurr Hos, Moses Mabhida, Mandera Bridge, Samora Machel, Osayiwaranso King Langalibhalele , Rhodes Dr

 33. Please can’t our leaders for once think of a different name? i.e Malawi International Stadium or maybe Lilongwe International Stadium. Everytime it’s Bingu this……Bingu that…… I think we are over commemorating him, think about this.

  1. palibe chanzeru walankhulapo apa wangoonetsapo umbuli wako. ukudziwa zoti kuli kamuzu stadium ku malawi kuno? ndiye uzifunse kuti inasinthilanji kuchoka ku chichiri stadium nkukhala kamuzu stadium

 34. tingofunsa nawo bwanji asatenga silver ndi bullets imodzi ya ku Lilongwe inodzi ya lumwela nanga sizikukhala ngati kuti ku Lilongwe kulimbe ma timu ?????

 35. Last of last month this ground is opened by chinese national team and malawi!! Now nyasa big bullets and manoma!!!!After that uwii here Bangwe stars and lilongwe hummers will open international ground• Nde atolakhani a malawi amenewo amangotola ndi zoola zomwe•Osamadandaula shoooooo matolakhani onse!!

  1. am from BT ndagwirizana nawe kukondera kwake kotani agalu amenewa anakatenga imodzi yaku bt ina yaku lilongwe osti zopusazo .

  1. Sizingakome popanda BULLETS baba,u can’t talk abt Malawian ftb without de ppoz team BULLETS kkkkkkkkk believe it bru

 36. aaaaaaaaaaaaaaaaah ma teamvosatha mpira ameneo……osayitana national team bwanj mesa ndi ground ya national team not those useless club who can’t pay a player 1 million per month

Comments are closed.