Ntchito ilipo pa mayeso a Fomu 4: ati a MANEB azifunsa kuyambila zinthu za Fomu 1


exams

Kuthetsedwa kwa mayeso a Fomu 2 kwabweletsa mavuto ambiri pa ana amene asiya kulemba mayeso amenewa.

Mavuto awa adza zitadziwika kuti bungwe loyang’anila za mayeso m’dziko muno la MANEB lili ndi ma plan oti tsopano mayeso a Fomu 4 azikhala ndi mafunso oyambila zimene ana aphunzila Fomu 1.

Malingana ndi chikalata chochoka ku bungwe la MANEB, mayeso a Fomu 4 tsopano azikhala ndi mafunso a zinthu zones zimene ana aphunzila ku Sekondale.

exams“Paja kale lija timangofunsa za Fomu 3 ndi 4 basi pa mayeso a Fomu 4, koma tsopano zinthu zasintha. Pano tizifunsa zones kuyambila za Fomu 1,” atelo a MANEB mu chikalata chawo.

Zimene a MANEB alengeza zadzetsa tsemwe pakati pa a Malawi amene ali odabwa ndi zilinganizo za MANEB.

Anthu ena amene ayankhula ndi Malawi24 ati zimene akukamba a MANEB ndi zovuta kuti zichitike.

“Koma ngati amavuta mayeso a 4 aja zinthu za Fomu 3 ndi 4 basi, ndiye akanene kuyambila Fomu 1? Apa ayi ndithu apaunikile bwino,” anatelo mkulu wina pothilila ndemanga.

100 thoughts on “Ntchito ilipo pa mayeso a Fomu 4: ati a MANEB azifunsa kuyambila zinthu za Fomu 1”

  1. i think this Dpp goverment is afraid of other graduates they want to maintain their current positions as far as education is concerned this government has done nothing apart from raising the tuition fee.For instance polytechnic students are just moving up and down pamapeto munthu akapalamura akuti pereka 3million nt only poly zomwe zikuchitika pa mzuni pamapeto timva aseka school.Malawians i cry for u becouse how can we talk about social-economic development if our children are at home roting with ignorance? this is not point of children working hard but this regime wants that iliteracy level should go higher so that akamayakhula chizungu tiziti inde bwana just becouse we can speak english what a pity!

  2. i feel very sorry for my beloved mother land(nyasaland)nothing is never been stable since when Dr H.kamuzu banda decided to let it go(died)today this and that !!!!,tomorrow,…. shit,here we go back again.simaphunziro okha,even vacancies,monga police, prison,Malawi army, teaching. amati tikufuna anthu 4 thousand, end of a day,anthu 3 thousand amakhala ana kapena zibale za mabwana.anthu 6 hundred odisha ndalama,the least 4 hundred akuti yathu imeneyo tinyosolelane,kkkkkkkk. do you think mphawi wa ku mudzi apa pali chake??? not only that, even ma research projects abwino amalembana okhaokha,ife timangonva atii kunali project ya(……)kunva zothaitha shaaa!!!….lero kuli atiii,Ulimi wa nthilira,one village one project, Green belt, atii Ulimi ya mtaya khasu hahaha….nde kutikodola zisanayambe ndi komwe,cholinga tizilima kwambiri kuti iwowo azidya kapena kutigula pa mitengo yotchipa.hahaha ameneyo nde malawi walero.

  3. i feel very sorry for my beloved mother land(nyasaland)nothing is never been stable since when Dr H.kamuzu banda decided to let it go(died)today this

  4. kusowa chochitatu uku,akulu akulu ndithu round table discussion,mataye kuno suti zili pholipholi kugwilizana zimenezi,ndiye chimodzi modzi wana kusewela pamchenga,hahaha malawi sazatheka.

  5. Ooh dat plan mu malawi zibwezeresa umburi wazaoneni bola zinthu zikadakhala ngati kale momwemuja bwanji dat system its not gud many pple will drop at xul 4sure

  6. Hahaha ..thats what i really 100% know about malawi ….though they will do that we dont given opportunities to work with that msce paper ..imagine ayoung person from malawi deserve to spend 16-18 years searching for better education after all he has all the papers from university umva kuti ulembedwe ntchito u must have 4-8 years experience ….rabish.where do we gate experience while you are not giving us opportunity …..marks zero MANEB

  7. Kufuna kuchulukitsa umbuli pa Malawi. I wonder what the government is doing about this mwina poti ma mp ambilinso xool yawo imakhala yo pelewera. Kodi nfundo imeneyi can’t be contested in a court of law????? This is just too much.

  8. Nanuso a Malawi24 mumasowa zopanga post eti? MSCE amafusa from primary to form4 ndie pali zachilendo apa? a Malawi Vomelezani kusintha dzulo silero mesa kale anthu amkalemba mayeso a boma mu std5? zilikoso lero? it was only Malawi left behind wth JCE, Osaopseza ophunzila MSCE izifusidwa mwa normal like mmene zimakhalira (Malawi24 unproffessional web pages) Muziposita zakupsa osati mbwelera madzala mphuno okhaokha ndi ufulu wanga kulankhula zakukhosi (SECTION 35)

Comments are closed.

Discover more from Malawi24

Subscribe now to keep reading and get access to the full archive.

Continue reading