Ntchito ilipo pa mayeso a Fomu 4: ati a MANEB azifunsa kuyambila zinthu za Fomu 1


exams

Kuthetsedwa kwa mayeso a Fomu 2 kwabweletsa mavuto ambiri pa ana amene asiya kulemba mayeso amenewa.

Mavuto awa adza zitadziwika kuti bungwe loyang’anila za mayeso m’dziko muno la MANEB lili ndi ma plan oti tsopano mayeso a Fomu 4 azikhala ndi mafunso oyambila zimene ana aphunzila Fomu 1.

Malingana ndi chikalata chochoka ku bungwe la MANEB, mayeso a Fomu 4 tsopano azikhala ndi mafunso a zinthu zones zimene ana aphunzila ku Sekondale.

exams“Paja kale lija timangofunsa za Fomu 3 ndi 4 basi pa mayeso a Fomu 4, koma tsopano zinthu zasintha. Pano tizifunsa zones kuyambila za Fomu 1,” atelo a MANEB mu chikalata chawo.

Zimene a MANEB alengeza zadzetsa tsemwe pakati pa a Malawi amene ali odabwa ndi zilinganizo za MANEB.

Anthu ena amene ayankhula ndi Malawi24 ati zimene akukamba a MANEB ndi zovuta kuti zichitike.

“Koma ngati amavuta mayeso a 4 aja zinthu za Fomu 3 ndi 4 basi, ndiye akanene kuyambila Fomu 1? Apa ayi ndithu apaunikile bwino,” anatelo mkulu wina pothilila ndemanga.

Latest vacancies

97 thoughts on “Ntchito ilipo pa mayeso a Fomu 4: ati a MANEB azifunsa kuyambila zinthu za Fomu 1”

  1. Hahaha ..thats what i really 100% know about malawi ….though they will do that we dont given opportunities to work with that msce paper ..imagine ayoung person from malawi deserve to spend 16-18 years searching for better education after all he has all the papers from university umva kuti ulembedwe ntchito u must have 4-8 years experience ….rabish.where do we gate experience while you are not giving us opportunity …..marks zero MANEB

  2. Kufuna kuchulukitsa umbuli pa Malawi. I wonder what the government is doing about this mwina poti ma mp ambilinso xool yawo imakhala yo pelewera. Kodi nfundo imeneyi can’t be contested in a court of law????? This is just too much.

  3. Nanuso a Malawi24 mumasowa zopanga post eti? MSCE amafusa from primary to form4 ndie pali zachilendo apa? a Malawi Vomelezani kusintha dzulo silero mesa kale anthu amkalemba mayeso a boma mu std5? zilikoso lero? it was only Malawi left behind wth JCE, Osaopseza ophunzila MSCE izifusidwa mwa normal like mmene zimakhalira (Malawi24 unproffessional web pages) Muziposita zakupsa osati mbwelera madzala mphuno okhaokha ndi ufulu wanga kulankhula zakukhosi (SECTION 35)

  4. koma szabwino, kuymbra primary mpaka scondary 4m 4 otsaziwa kuynkhula english. amen apangzimenezo potzao zidayenda enafe mmmmm kulilabac.

  5. Boma-la-democrancy-eeeee-padziko-lamalawi–palibe-chomwe-chizamange-malawi-wabwino-mumabweretsa-ndondomeko-ngati-mukufuna-kukonza-koma-kulikuononga–kamuzu-adatsogolera-dziko-lamalawi-pofuna-kwathandiza-amalawi-pamaphunziro-kare-wa-standard-4-amalankhula-chizungu-lelo-mpaka-form-2-ena-chizungu-kulephera-chifukwa-chiyani-Akuwunduna-wamaphunziro-zambiri-mwakwefulakwefula-kodi-mukufuna-akutameni-poti-ndinu-zanu-zidayera-kare-?

  6. Very sad. After 52 years of Independence authorities in the ministry of education have not yet explored the standard curriculum for high school students.

  7. Ine ndimayesa mutiuza kuti mayeso abwelere a standard five koma mukuthesa jce ukunama iwe wazipeza zimenezo zizabwelera!kumbukila mchimwenewako za flag inabwelela !
    Anyway ur moron stupid chavumbwah President

  8. ngati work ya 3 4 ana amalakwa ndie akaikenso 1 2 zoona? kodi dzikoli likupita kuti? ndani ochuluka nzeru akusocheretsa anthu anzeruyo? dzuka malawi dzuka

  9. POYAMBA AKALAKWA A4 AMABWELEZA AMAYAMBA M3 NDIYE PANO U MIN KUT AKALAKWA AZIYAMBASO MU 1 OR W? JUST STUPID POOR PPLE%

Comments are closed.

Discover more from Malawi24

Subscribe now to keep reading and get access to the full archive.

Continue reading