A polisi m’boma la Salima ati akusakabe yemwe adapha mlaliki odziwika bwino mdziko muno a Shadrek Wame.
Oyankhulira a polisi m’bomali a Gift Chitowe ndiomwe anena izi dzulo lolemba pa 31 Okutobala.

A Chitowe ati iwo anakhazikitsa kafukufuku ofuna kugwira yemwe adachita chipongwe chimenechi ndipo anaonjezera kuti pakadali pano kafukufukuyu adakali mkati.
Mneneli wa a polisiyu anatsutsa mwantu wagalu mphekesera zomwe zikuveka zoti iwowo agwira yemwe akuganizilidwa kut anapanga chipongwechi.
Iwo ana izi sizoona ndipo anakanaso mphekesera ina yomweso yaveka kuti munthu oganizilidwayo anaphedwa ndi anthu olusa mdelaro. A Chitowe ati zosezi ndizabodza.
“Ife a polisi tikufuna titsutse mphekesera imeneyo chifukwa palibe yemwe wabwera ndikutitsimikizira kuti yemwe adapha malemu a Wame wamangidwa kapena waphedwa ndi anthu olusa, choncho zosezo ndizabodza. Chomwe tikudziwa ife ndichakuti kafukufuku ofuna kugwira yemwe adachita chipongwe chimenechi adakali mkati.”
Atelo a Chitowe. Iwo aonjezera kunena kuti anthu osiyanasiyana akuwatsina khutu momwe angampezere nkulu yemwe adachita chipongwe chimenechi.
Mlaliki Wame adapezeka ataphedwa mnyumba mwake mmawa wa la chisanu pa 28 Okutobala.
Ma lipoti akuonetsa kuti malemuwa adaphedwa ndi wantchito wawo yemwe adasemphana naye chichewa pankhani ya chimanga. Malemu a Shadreck Wame adabadwa mchaka cha 1940.
Iwo ankachokera mmudzi wa Mwanzalamba, mdera la mfumu ya ikulu Kambalame m’boma lomwelo la Salima ndipo aikidwa mmanda dzulo lolemba pa Okutobala 31.
67 thoughts on “A polisi akusakabe yemwe adapha mlaliki Wame”
Comments are closed.


Akapezeka Mateyala Anyeke Paiye!Ndimoto Wa petrol Basi palibeso Zokambilana naye.Ndinyumbayake yomwe Tikayatsa Aonaso!!
IN JESUS NAME KAZIPELEKE WEKHA PASANATHE MASIKU SEVEN. Ukachedwa uzikhweza wekha.
Chiwanda Choipa Chimuzungulile Apaali.
We need to show love to one other.This preacher was not supposed to die like that and i was shocked to hear that.Please police do you your best to arrest the suspect.MHSRIP.
Munthu anapanga zimeneziyu Chauta apange naye. Abale inu….just this same year mwana wao yemwe amawathandiza…he was residing here in South Africa…anapezekanso atamwalira mu bedroom mwake….sort of like anachitanso kuphedwa…in broad daylight. Mpaka pano his death still remains a mystery. A few months down the line….Bambo akewa also gets killed in such a brutal manner. The late son left six children who were apparently being taken care of by agogo awowa.
Its so painful. May the Almighty Father God intervene…more especially kwa anawa. He is the only one who can take care of their welfare.
LET HIM COME BACK AND EVEN SAY SORRY TO YOU.
HERE IS HERBALIST AND TRADITIONAL HEALER TO HELP YOU..+27725564721
Are you depressed ,feeling disappointed by your lover that he is changed you nolonger understand him any more then here is Herbalist Healer Shamim to help you flash away all those that are after him…
Do you have any one prisoned but you want him be bailed out then come be helped,Are your kids not listening at you make them listen and understand you or be at good terms with them
Am good in
Bringing back lost lovers
Stop Cheating and Breakups
Flash away all those after your lover
Students Pass Exams
Bringing Back lost or stolen goods
Iskhafulo or sea water
Stop divorce
Come for my manyonix Man power for your man hood
Is any one hating you at work stop that
Make your boss like you
Get promotion at work
protection spells to protect your properties
Lock heart of your lover not to love any one else
Ubheka mina ngedwa
Remove or put iscitho
Stop family misunderstandings and fights
Come i cleanse your home
Are you having Bad dreams come be helped
Make your lover marry you and do as he promised you
Are you having haunting spirits in your home i remove it away
Make your lover feel you and get satisfied of you in bed
Lock heart and his man hood be yours only.
I have a cream which can make your penis big and strong permanent.
CALL or Whats app +27725564721
Amalawi24 simumatha kulemba nkhani mungokhala musamalembe
Apange zimenezo kaya, Mulingu awathandiza
Munthu ameneyu agwida ndithu. Mulungu wa mphamvu amusaka munthu ameneyu mpaka apezeka. kukapha munthu wamkulu ngati ameneyu kuti iye apezapo chiyani?
Apa Osanyengerera Munthu Ngati Apolice Samupeza Ayenera Kukayankha Mlandu Wopha Munthu Chifukwa Nditchito Yawo Yofufuza
mvuto ndilakuti amalawi timalemphela kunena zoona potelo apolic amatenga nyengo pakafukufuku pakuti athu oipawa amadisidwa manyumba. koma kubukani kt mulungu salemphela patalike bwanji adzapezeka
Munthu oipayu akuyenela kulangidwa ndithu akagwidwa,wapha munthu yemwe adali okondedwa kwambiri ndi anthu ndiponso mtumiki wa Mlungu yemwe amagwira ntchito yake mosanyengelela munthu koma kunena chilungamo.tamuikani nkhope yake pa Facebook kapena ma newspaper kuti timudziwe kutheka timakumana naye koma kamba kosamudziwa timangomudutsa
Mzimu Wanu Ukause Mwa Ntende,
How far he can go the world is round
Nzimu wa mlaliki wame umusake munthu ameneyu, nkhosa zosochera zambiri awame amayenera kuzilondoleza kwa atate kuzera mumaulaliki decemberyu. Mphambe achitepo kanthu.
Munthu wa bwino akutumikila ntchito ya mulungu aaa apolice yesesani kugwila ntchito yanu
Koma abale iiiiiii kupha munthu anakulakwilani chani
Apolice Athu Tisawanyoze.Chfukwa Murder Case Siyoenera Kuitenga Mwachbwanabwana Ai..Tieni Tikhale Pheee Afufuza Mpaka Munthuyo AMugwra..Tien Apolicewa Tiziwapatsa Mangolomera Osat Mphwayi..Tiziwafunira Kafukufuku Opambana..
Hahahahaha ask for help from FBI in simumupeza mazoba
What going around comes around God is after him.
Dear Influential Individual, We are delighted that your life’s journey has led you to discover our organization. we value anonymity. We see and know all just as a shepherd sees and knows all of the flock, our eyes peering over the masses to identify any threat. We are the bringers of new dawns, the guardians of the human species. We are the Pyramid, the Eye, the Light, the Eternal. We are the ILLUMINATI. The ILLUMINATI is a collective of prominent figures throughout the world who have united to guard the human species from extinction,we create wealth and make our member famous and rich in their own line of work. Our members bear the burden of a planet’s leadership with the lives of 7 billion in their hands. As the human continues to rise above its other animal counterparts, governing of the planet has turned into a daunting task. In return for their loyalty, our ranking members are presented the opportunity for lives of limitless wealth and opportunity. Once a member, the requirements are unimposing and often spaced between many years. Our requests are simple and therefore may be hard to comprehend, but disloyalty is not tolerated. You must understand this before applying. Members must fulfill their oaths to the Illuminati under every circumstance and recognize that they are merely one part of a much larger Universal Design. For centuries, our organization has separated individuals of outstanding political, financial, or cultural influence from the flock, and established them as shepherds of the human species. Perhaps you have already proven yourself in these fields. For that, the Illuminati officially congratulates you. Your dedication gives hope to us for the future of the human species. If you would like to continue your application,and willing to pay a sacrifice start by reaching us on my facebook account JOHN FRIGHT and you will be added to our list of potential candidates for Illuminati membership,and you instant reward will be given you on the first meeting sincerely.