Mutharika criticised for failing to attend Gwanda Chakuamba’s Funeral

Advertisement
gwanda-chakuamba-funeral

Malawi President Peter Mutharika has faced criticism over From some quarters for his decision to shun the funeral ceremony of the country’s Veteran politician,Gwanda Chakuamba,who has been laid to rest on Friday,October 28,2016 at his Zuwere Lodge in the area of T/A Mlolo in Nsanje.

The concerned people said although Chakuamba’s funeral was honored with full military respect,it was necessary for Mutharika to be in attendance at the ceremony and no delegating his minister on such occasion.

gwanda-chakuamba-funeral
Mutharika did not attend Chakuamba’s funeral.

President Mutharika was on this day been represented by Minister of Agriculture, Irrigation and Water Development Dr. George Chaponda which brought mixed reactions among people.

Among other notables faces that were seen at the ceremony of late Chakuamba at Chinyanje Village includes: former President Dr. Bakili Muluzi, MCP President Dr. Lazarus Chakwera, John Tembo, Moses Dossi, Speaker of Parliament Richard Msowoya, Deputy Speaker of Parliament Esther Mcheka Chilenje Nkhoma,Cabinet Ministers and his best friend,Bazuka Muhango SC.

The Lower Shire valley political giant, Gwanda Chakuamba died on Monday while receiving treatment at Blantyre Adventist Hospital (BAH),after succumbing from chronic diseases such as heart attack among other illnesses.

He died at the age of 82 and has been survived by a wife,Raima,Three children,Four grand children and three great grand children.

Advertisement

395 Comments

 1. Hahaha following. Mungolimbana za ziiiiiji. Wina ali mmanda may he RIP wina pa king size bed with an air conditioner. Olo zoti its hot they both dnt knw inu mukumva kutentha. Ur busy kulimbana. Malawians let’s focus on important things pilizi. Mwapindula chani. Kaya walakwa peter kaya ayi mwinaso sakuganiza. Kkkkkkkkkkk

 2. take t easy I am sure Pitala adzapezeka zikatigwera enafe

 3. ask his relatives,they will tell how cruel monster apm is.he doesn’t even go to funerals of his own relatives and you expect him to go to gwanda’s funeral.

 4. ANYTHING Called “ISM” is evil and belongs to hell. Criticism, satanism, humanism and the rest of the isms. no need to practise the isms in as far as funerals are concerned because if my memory saves me well i never liked to go to funerals for show, appease, please anybody or fear anybody. moreover funerals are expensive and a drain of hard earn resources. i would rather support the idea of putting resources over prevention of sickness and healing. “chotsa chipika m’diso lako kuti upenye bwino, nkuchotsa katsitsi m’diso la m’zako.”

 5. Peter don’t care about Malawians so don’t surprise if something like this happened, what u gona hear every time is ;his supporters defending him

 6. So He Not Supose To Make His Own Disitions Coz He Is President, What Could We Benefit From That, Lets Think About Development Than Westing Our Time Speaking Useless Things. He Have Rights Like U And I

 7. Even though you can back up errors with our leader, am also concerned he was supposed to be there,palibe chotukwanilana, he Iz the head of leaders in this country, must be exemplary, apa apita ku idol worship mulhakho wa Alomwe! Dr Muluzi was on forefront @burial of veteran Chakufwa Chihana, see Aleke Banda, he was there too, tsoka ngati zolakwisazi zamchulukira, rem amati tsoka likalinba umakuotcha ndi Nkute, a Bwana ndiwowasatira must change in decision makings, truth pains, let Malawi feel we have leaders with humility, anyway Madzi akatayika sawoleka”’Voice of voiceless Malawi ‘

 8. Kodi mtundu wa a Mutharika ndi anthu? They are full of thweselves yet they claim to be Malawians. Which Malawian can be as cultureless as these idiot? Where did they study after all? Kamuzu tuaght us to follow our own culture that marks us different from other countries even in this african region. Nobody knows when to die or when such thing befalls us, zikachitika munthu amasiya ma program ake onse ofunika just for some hours and concetrate on the funeral.
  His brother also dispised Chihana funeral by sendind the same Chaponda, buros, macacos inculturados, educated cultureless savages. Nao tem vergonha? Very shameful leaders.
  Thanks Dr. Muluzi you are such a humble guy even when you were in power not these fortune seekers, good for nothing feios, cara parece ante-passado Peter Mutharika.

 9. verteran ndekuti chani,amalawi tamanenaniko zowona.sujatimkava kwa amuluzi kuti gwanda chakwamba munthu oyipa,nangalero mukuti chiyani.mulakho woyeeeeh.

 10. MMMMMMMMM MALAWIANS PLIZ PLIZ PLIZ TIYENI TIKAMBE NKHANIZI MWANZERU KUPITA OR KUSAPITA ITS ALL THE SAME..MMENE SANAPITEMU NDEKUTI GWANDA SANAIKIDWE MMANDA?

 11. Thats much of what we had been saying of mispriorities, SO HE IS ATTENDING MLAKHO WA LOMWE AND FAILED TO ATTEND GWANDAS FUNERAL? What development does Mlakho bring to Malawians? And you can read down some of the comments of some poor thinking upsided minds still backing him as if they are telling the truth. Guys if your minds has gone crazy because dpp fed you at one point in time or cashgate has driven you mad, leave the commenting platform to those who are principled. Poverty has changed you to ihuman and you look at dpp as your saviour. THIS DPP IS A WALKING DEVIL, JUST IMAGINE BUYING A NEW FLEET OF CARS IN TIME OF HUNGER, GOING TO MLAKHO AND FAILED TO ATTEND GWANDAS FUNERAL, ETC, THIS DPP IS A SATAN AND WILL FINISH US IF WE CANT CHANGE. LETS BURRY THIS DEVIL ONCE AND FOR ALL. THE BALL IS IN OUR HANDS MALAWIANS, LETS GO FOR THE TRUTH AND BOOT OUT THIS EVIL PARTY.

 12. kkk koma my mai mw bwanj kod? akanaptaso munakapezabe conena, peter amakanyadisa galimoto ku maliro.peter akuwononga ndalama za boma,anatenga anthu 100 kumaliro.

 13. Ndawona anthunu munali ndi zolinga kuti mukampase mphepo yoipa enanu ndawona munenera chibwana mwina simuziwa zomwe zimachitana andale kuti pano even ufumu wakumuzi ndiwowopsa kwambiri ngati ukungoyenda za wamba chilipo chilipo inu simungaziwe mwachepa ngati ndi chibwana muzaona polekela ndi mkulu uyu amayenela kufufuza asananyamuke

 14. Zachibwana, pali mau mu baibulo oti musalile one Koma muzililile inu ndi ana anu (mwana wa mulungu anatelo). Mulimbana ndizinthu zoti inu simungapindule ngakhale pang’ono olo akanapitako ndiye kuti mavuto athu akanatha? Ming’azi.

 15. #Doreen &#Agie kodi mumadziwa ulendo wapresident yekha is cost millions kwacha president ngati sanapite kumaliro is not a case president amapangila maulendo samayenda ngati iwe ayi malawi ndi dziko losaukitsisa padziko lampansi chifukwa mwina akanapita akanawononga ndalama zambili

 16. Kale kale kumaliro timadyako nyama,nsomba za matumbi pano kumaliro kukumakhala bonya otendera ndi cabbage nde Mumati Muthalika akataniko? Sorry akudwala nkono ukumuvuta saaaa

 17. Mwagwa nayo tiapitafe sitinakwane ,mukukhala ngati amayendera ndalama za ZBS ndi MCP ku chipatala cha ku India ndi SDA HOSPITAL BWA,

 18. Mwagwa nayo tinapitafe sitinakwane ,mukukhala ngati amayendera ndalama za ZBS ndi MCP ku chipatala cha ku India ndi SDA HOSPITAL BWA,

 19. Hahahahahah veteran ndiye ndaniso, wangofa ndi fungo la u president osawununkha nkomwe mpando, Boma sizibwana raaaaaa

 20. Failling to attend gwanda’s funeral does not mean that he dont know what he is doing, deffinately he send some people there representing his ruling. What nonses are u talking about? He is a president he has got alot of things to do 2019 – 2024 vote ndiyanu bwana

 21. Kupita kumalilo sitichita kukakamizana ayi ngati bwanawo anari ndizochita zina sichifukwa anthu inu ngati ndinsanje abale lekani siimanga mudzi lekani bwana agwire ntchito komaso muzilingalira mutakhala inuyo mungamamve bwanji? Mmmmm Malawi dzuka Malawi

 22. Mmmm dzuka malawi dzuka lija nd kale unayamba kugona,mmmm kod peter akanapitako ku maliloko gwamba akanauka? Wake up ladys an gentlemen,kod mukundiuza kut sanatumize nduna inailiyose yokamuimilila ku mwambo wa malilowo?

 23. #Ndye_akanadzuka Gwandayo?

  Mumafuna azaikataniko munthu ot mumkati wamwalira?

  Millitary order imene anapereka siikukukwanirani?

  #chabwino ndi chani mungakambe cha #President?…..chonsecho inu ndiazibale anu omwe amakukanikani kuathandidza.

 24. Chatapu mdzika yoyamba ku malawi ndi iyo kumatsatira enafe ndiye iyo amayenerera kukhala munthu woyamba kukhalanawo pa maliro agwanda osati zopusa zanuzo koma ndinu amalawidi mwaiwala zomwe mumachita kumudzi kwanu mfumu imakhala yoyamba kulira ndi kutsekurira kumanda adzukulu icho ndi chikhalidwe chathu ife akumudzi ine monga mwana wa mmudzi ndikuti akuluwa amayenera kukhanawo basi chemu

 25. This page wish too much politics. I am not a politician,I was wrong to like this page. I thought there will be entainment,education and informative.

 26. A Mw24 Sometymes simumakhala serious mukamalemba nkhani zanu..Mwakhala mukulemba zambirimbiri zokhudza Peter nd now mukut sadapite kumaliro,mumafuna akapita kukapepesa muzatiuze kut”walakwitsa wapepesa ndi ndalama zambirimbiri yet anthu akugona ndi njala”shame on u AGANYU INU.

 27. peter is a public figure.enanu kaya munapita kapena ayi,palibe angakambe za inu.palibe amakudziwani.malwians need a presdent who can read by an examples.pipo didnt c him kumaliro kwa gwanda chakuamba,a veteran politician that any malawian knew and respected him.that is y maliro ake analemekezedwa.ndie if pipo are pointing bad things from their presdent enanu musamasokose.bring mfundo timve kwa inu.

 28. Mtsogoleri azipita kumaliro pamenepo ndipamene amadziwika kuti uyudi ndi mtogoleri. komabe investigation ikhoza kuthandiza, kuti tidziwe chimene chinachitika. Pepani a President a Malawi, muzipita mmaliro azanu.

 29. wat iam saying rytnow iam Nat gonna change I will and say it again,,,the #Mutharika they are realy blessed wit Loyalty family yes,,,but they are very very stupid both even his late brother he was also stupid,,,:how can u do DAT,,,Waiwala kale kuti amafuna kutfa iyeyo mkuthawa amalephera even kupanga adress anthu Ku #Lilongwe and now u are failing to go there ??the fact is mumatha kuyamba zinthu koma ubwino wake mumafa msanga nawo mantha coz mutharika ndumuziwa ine tikazayamba kukokana naye NkhAni ya NdalAma zaBoma ndakaika ngati azatha kuyankha

 30. i have always maintain my opinion that peter is the worst president malawi has ever produced,this old stupid guy doesn’t have quality of learship,he is arrogant and i really don’t comprehend why some pipo voted for him.try to listen to his speeches when he is talking to my poor fellow malawians,he doesn’t know how to speak properly any malawian langu,oooh my God pls help with a good leader,how could he not attend the funeral……..!?this old man is destroying our country he must go back to america pls….my heart is really soul,i hate this old.

  1. point of correction. u could hv used every malawian nt any malawian, the nxt word correct it urself. nw evn if doznt speak properly but he cant speak ur broken english. 2) GOD created him & put him there or r u judging the creation of GOD nt wat u r saying? be careful 4 u dnt knw may be ur kid(s), relative, or urself may meet smting more than that pangozi mkudzakhala osayenda, osaona, osabereka so u can talk anyting but nt the way he woz created.

  2. your english grammer is so poor that i can’t comprehend what you are saying pure,you talk like your stupid president peter,there is no point in your long and boring statement pure.

 31. koma nde kulimbana ndi president aah fuck off apumira pati muthu, chilichose basi kumango kamba zambiri…haaa za galimoto lexus apa mukut y sannnapite kumaliro and last tym it was about USA;; mwabowa

 32. Nsiyeni mbuya ause muntendere.or evn Apm akadaendako mbuya bwenjimbo alamu ka? ?nkhabe. Tayu waenda waenda anajatifunambo weneyi 2019 ndichinchinobi

 33. Ngati mukusowa chonena just b quite zot amakupatsan ndalama tizitaye uko this is serious issue…munthu yemwe akutsogolela dzilo azikhala good example. Amayenera kupanga attend bas kumangowabakra chlichose bwanawa sasintha ata

 34. palibe vuto pakusapita kumaliro kwa gwanda,monga tiziti sanatumize nthumwi?kapena tiziti mtembo wakana kulowa m’manda poti peter sanapite?pezani zina zokamba.

 35. Inuyo chakuyabwani ndichiyani? Kodi ulemu wake mmafuna iye akakhale mdzukulu wakumanda? Guys lets be serous with developing our country rather than sayng nonsense things. Gwanda was an opposition veteran politician so wats wrong with you?

  1. I think its common sense needed. Attending and being undertaker (mudzukulu) are 2 different things. Being opposition does not mean u are enemies. Thats is multi-parties democracy? Do u mean when Bingu waMuthalika passed away they was no opposition leaders at the funeral? What masage are u teaching youth? Its about (uMUNTHU). I think we need civic education to understand much better democracy. He was suppose to lead by an example that he love everyone no matter we have different political parties,views,religious,tribe,age what so ever that we are all Malawians. Shame.

 36. Apatu sinduwonapo nkhani yoti mmpaka. Kwawoso anthu akakafa inuyo musakapite basi tee nkhani yatha apa ndi mmenetu amapangira ku muzi kaa. Umunthu a Malai wabwera poti wamwalira ni. Gwanda kodi? Uja mumavina dance nkumamwwa wine Bingu atafa. Uja mumakambirana pa wayalesi mumati Zodiak za matenda a munthu komaso maliro kulengeza ngati mpira. Musiiyeni APM dikirani nthawwi yanu muzikapita maliro aliwose kaa mwinaso inuyo simunapite ku maliroko koma munali ku Nsanje.

 37. Surely he can not be all over and everywhere more especially after the gruelling trip to Mchinji on Thursday ahead of another trip to Mulanje on Sunday. You agree with me those of you who have studied management that a good Manager is one who delegates, its in the bible, ask Moses

 38. kupereka fulĺ miltàry honour kwakuchepeŕàni .peter akanapitáķo omutsàta akanakhaĺa angáti? ndaĺama zikánáoñongeka zochuluķa bwànji?think be4 speáking

 39. Ineyo chomwe chimawavuta akuluwa sindimadziwa kuti ndi chain,ndakhala ndikupita maliro ambiri aanthu andale koma nkulu ameneyu osamva kuti pabwera a president,iwowa being first citizen amayenera kukhala chitsanzo,akanakhala wina akanatengera chitsanzo chabwino cha a Muluzi former president,maliro ambiri omwe anthu ake amakhala ma top gvt officials a chair amakhala ali konko,ikafika nthawi iyi ndale kumasiya Kaye uko bwana,olo zitakhala kuti munthuyo umadana naye koma nthawi yokhayi zimenezo kumasiya Kaye nkupanga attend maliro plz plz,I was there yesterday,people were very happy to see atcheya,komatu ngati ndi ma adviser bwana,amenewowo awonjeza ndale kwambiri,tisaiwale chikhalidwe chathu cha chimalawi.

  1. One thing that is making Malawi unproductive is this tendancy of going to every funeral that happens. Uwona office yonse kutseka akuti apita ku maliro a sister wawo wa akazi abwana mamuna wake! Counter productve and waste of resources, ngati chili chikhalidwe chithe!

 40. know that he’s someone who doesn’t move anyhow,there are alot of factors to consider before the president attends any event.it can be security or financial problems which cannot be announced in public.so just be silent because you dont know what was going on.

  1. Zabodza izi,first citizen needs to be examplary,despite whatever facts,security yake iti?kuli chani Ku Malawi kuno chopereka threat kwa mtsogoleri Wa dziko?

  2. Komanso munthu ukakhala kuti sunabeledwepo chifukwa cholembera mulonda sumachiwona or kuikitsa ma burglar bars umakutenga kopanda ntchito, ndiye uzakati chitetezo chake chotetezera kumalawi kuli chani choopseza, ndiye umbuliwo umenewo. Kugunata.

 41. Munatchera kuti mukamuwazire powder wanu uja kumeneko? Tidaletsa zimene zija. President asamango upita pali pose. Kwachuluka satanism ku Malawi. Anthu akumapoperana phundabwi pa maliro. Mu tchalitchi, pa whatsapp, pa bridge, pa chitsime, ku thobwa, mu botolo la green, ku phwando, ku ukwati ndi ku party. Chenjerani anthu opatsana nawo moni. Makamaka ngati ndinu nduna, MP, Governor, chief excuitive, manager, director and leaders. Osalora uima pali pose. Malawi yaipa! Anthu akuyenda ndi mabotolo mthumba. RIP Gwanda!!

  1. Chimene chapangitsa kuti iwe ugwiritsa ntchito dzina labodza ndi chani? Sindiye ufiti umenewu? Kuti usaonekere poyera! Ukuopa chani? Bwera poyera tive.. usabise dzina. Yasmeen Alice Ndemboh

 42. Andalale mwatokota kwambiri koma nanga akhristo tikuti chiyani Za Wame nayenso sanali munthu wamba pufunika ulemu wapadera …….Tiyeni tiwachititse manyazi Andalewa tigwilane manja polemekeza munthu wamungu

 43. Chisoni ndi kumatenda kumaliro ndi chikhakhali. Inu mungasankhe chiani (1) kukuthandizani pa matenda
  (2) kudzakhala nawo pa maliro anu.

  Tiyeni tizidandaula zothandiza dziko. Paja amati ‘ the 1 wo is quick to blame is lame.

  Wolira wenix2 ndiuti
  (1) amene waluza chuma chake pofuna kuti achire ndi
  (1) amene wasambasamba ndikukakhala pa mwambo wa maliro nyang’a

 44. This is unfair !!What kind of a Person is this one ?Timakhulupilira kuti Mtsogoleri amapezeka pofunika kupezeka ngati pa Maliro a anthu ofunikira ngati amenewa.Iyeyu sadzamwalira ?Sipadzafunika anthu ena ngakhale azipani zina ??This is Furish things !! Ican’t Tolaret this nustry behavior Tell Him !!!

 45. MMMMMMMMMM

  Komadi abwino sakhalitsa……
  ndaonera frozy .

  Zoona kusiya
  Black punch,
  Tripple X,
  Win,
  kachasu,,,
  kadansana,,,,,
  Delunde…

  Zonsezo kuzisiya
  Nkukachotsa Frozy???!!!!

  Frozy analakwa chani Frozy abale inuuu eeee???!!!

  Ndalira mokweza ineeee………

  Ndipo ndatsimikizano kuti Petter nde basi sadzathekanso mpaka ku Ndata ooooooh,,,!!!!

 46. mwasowa zolemba eti?Kapena muyetsa upresident ndi ufumu ndi ofanana eti kapena mumafuna akapitako mukamukonzere komweko mwalemba madzi…..Viva APM

 47. if he is lacking pasion to his fellow southen region pple what evil should pple of Northen and Central region expect??? An arrogant old man who only hears what his brain is telling him..An old man who only fill up his pockets…An Old man who is busy buying expensive cars when his pple are suffering…An old man who doesn’t even spend asingle minute of his night thinking about poor pple of his country…An old and economist Man who found out raising Taxes is the only way of improving the country`economy…Let my brothrs n Sistrs describe u again below…

  1. No need to ask, its written all over his face that he hates northern region. We are just surprise that he hates also other pple 4rm southern. Tribalism and nepotism.

  2. Are you talking of the very person you said was dead? Waukano and ur blaming him of buyin a car? Parliament passed abudget of the state to buy 8 vehicles on his convoy & yet ur here criticising him of just buyin 1 car out of the 8 parliament approved? Where were yu the time the budget was passed? You shld’v blamed the MPs 4 approving that budget not the fulfilment of whats already in the budget..

  3. sm ppo wl accuse u though u r nt doing anythng wrng. ths iz nt an issue if u gt nthng to say b silent rather than just talk, u wl end up syng nosense lyk saying someone is dead while he’s nt.

  4. the president did nt rise tax but the parliament did and if the parliament wasnt wiling it could nt hv aprove. so wat r u saying?, the president bought 1 car instead of the 8 aproved by the parliament, so wat r u saying?. kumazitsatu ndi bwino osamangoyankhulapo.

 48. jst abt a wk ago munat muthalika sali bwono (akudwala) nw mukut muthalika sanapite kumaliro, hw many muthalika do we hv, gyz u ‘ve 2b crous wen doing thngz

 49. Ena alibuzy kulandira ulemelelo waziko lapansi kupita zipatara zakunga zipatala zabwino pomwe awame akulandila ulemelelo wakumwamba nziko kuchita kuwampa malilo kuchita kwaika garimoto yonyamula akuba ndizina zotelo chosangalatsa ndi chakuti zadziko ndizotsala bora zakumwaba

 50. Mwina mkono wayambilanso.Oh too bad.Komabe akanatha kumwako ma aspirini athuwa kenaka nkupezako bwino then proceed to attend the funeral kapena?

 51. Zazii,,,,tili ndi mavuto ochuluka muno mwamva,,,kupita kumaliloko sizikanatipindulira kalikose,,,,akadapita ndiinunomwe amene mukanamawelengesera ndrama zomwe waononga apa,,,,,

  1. Iwe Banda Akamalankhula Pa Ngati Apa Uziganiza Ndimavuto Ati Amene Mwatha Kuwachepesa Ndarama Zathu Mwathera Ku Amereca Ndiye Pa Nsanje Mphopapa Ndinu Mkuyipisa Presedent Adyeranu Uziganiza Iweso Ndiwe Maliro Ngatiso Ine.

  2. Ndaganiza nchifukwa chake ndayankhula,,,,,,amalawi mumakhala ndi chidwi ndi nkhani zopanda ntchito,,,,,pompa iweyo ukudandaula kut ndrama zaonongeka kupita ku america nde ukudandaula zoti sanapite ku maliro,,,,,ukuziwa kuti president amaononga ndrama zingat pa convoy yake akayenda?,,,,,_zinaz zmafnika kungoyang’ana kusapita kumaliloko ndekut anali ndi zofunikira kuchita zoposa malirowo

  3. Malawi akulephera kutukuka coz anthu ake amataya nthawi ndizinthu zopanda pake pali nkhani APA mawa muzilira kuti mukufuna chimanga cholandira zomvetsa chisoni

 52. Inu Nomwe Mukumati Peter Wamwalira Ndiye Mumafuna Lero Mukuti Sanapite Kumaliro Mwazindikila Lero Kuti Ali Moyo?

 53. Akayenda Mumati Atha Ndakama Zopandantchito Akalephela Mumati Sanapite Koma Inu Muli Ndi Vuto Komanso Achita Bwino Osapitako Chifukwa Akanatha Ndalama

 54. Inu nzeru ndi umunthu wanu umaonekera pa maliro basi? Ithink u and our president ,amene akusowa umunthu ndinu munapita kumaliro! Bwanji mutamva kuti APM anatumiza Gwanda ku chipatala bwanji simunatidziwitse ! Kodi kumufunira nzako zabwino pomwe akudwala ndikupita kumaliro chabwino ndichiti?

 55. What kind of leadership is that? In times like this we put our political party difference away. And stand together as one Nation. This was a good time to show Malawi that even we have different political parties, race,tribe,age, what so ever we are together. Tribalism and nepotism is damaging our country. Being in another party does not mean we are enemies. We are all Malawians. That is a democratic nation. We have different opinions and views but we are not enemies. What lesson is he teaching our youth. Shame

  1. As u said u are youth, that just tells me how premature u are. I dont think yo father can think the way u think. Just seeking attention neh. That total stupid for any elder to think like a std 1 kid.

  2. shame on u 2 for nt c wat the president has done to honour gwanda there. hu do u thnk authorises asilikali kukapanga perfome there?, mesa ndi president or do u thnk they jst done own there own?. iweyo ngat sudzipita kumalilo coz peter sanapite kumaliro a gwanda ndiiweyo oat ma youth. the youths got there elders to teach them morals nt the work of the president or do u tel ur kids to learn morals frm the president? kkkkk. some ppo ine

  3. I think its difficult for a crab to teach the young ones to walk foward when it walks sideways. Akanati kuli kulandila degree yaulemu, i am sure ukadaona kuthamanga. When he attend celemony, he use it as a campaigning platform. So i know kuti it was not going to happen at this funeral that why he chose not to go. Pty in Africa he is 3rd 4rm last clueless leaders we have currently.

  4. thats the problem u judge someone on ur assumptions nt on wat is hapening. r u saying o u hav writen its because u were thnking if it woz a graduation ceremony he wud hu been there? comeone talk on the hapenings nt wat u thnk could hv hapened.

  5. Francis i think u are not matured enough to have (UMUNTHU) by our African culture and tradition. Are u telling me that if it was someone in this Dpp he was not going to attend. I know that the President has a diary which he has programes and timetable. He stay long in America and he has to postponed his diary eg launching of IDs. Lets not run away from the facts. I wil give u few good examples of Muluzi he attend Kamuzu’s funeral, but Kamuzu was Mcp. He attend Chihana’s funeral but Chihana was Aford. Just to mention few. This president is selective even Traditional celemonies. Lets wait and c campaigning time he wil come and dish out false promises to those place that today u say he is busy. Programes are planned by pple and they can be change by pple as well. Hope he will vote himself and u who dont c that the ship is sinking. However even he leave or not zanga zinayera without effort of this goverment. I just feel for those blinds who wil keep working for us.

 56. Wazolowera kwa azungu munthu yu maliro timaika wikend osati nkati mwa wik timakhala tikugwira ntchito ndiye sizokakamiza,akanapitaso mukuti wapita ndi anthu ambiri akuononga ndalama.

 57. Inu a Malawi 24, nthawi zonse mumalemba nkhani zomwe mwaona kuti ndizolakwika,mutapanda kutero new yanu sidzayenda malonda, inu mumakhodza zonse zomwe mumalemba zimakhala zoona pamaso Mulungu, Anthu oyipa inu kwambiri

 58. Ameneyu tiyenera kumufufuza kuti ndimmalawidi chifukwa khalidwe limeneli likupitilira losapita kumaliro. Mmalawi ndimuthu wa khalidwe ndiokhudzidwa wina akamwalira koma peter simmalawi ( ndiathu ochokera ku mass)

 59. Komadi kunena zowonadi apa tiyenera kumalemekeza chikhalidwe chathu.Mnzako zovuta zikamuonekera tiyenera kupita kukakhalanawo pazovuta zake chifukwa mawa ndine ndiwe ndiye plz Mr Prezident muziteroko.Panopa tikutha kusiyanisa kwakukulu kwambiri iweyo Peter ndi nkulu wako Bingu.Kunena zowona Nkulu wako sungamufikile kutalitali kwambiri.Bingu anali modzi wopita kumaliro ndimakumbukila Mfumu Chikowi waku Zomba atamwalira anapita kukakhala nawo pamaliro ake kusiya nyumba maliro a Mkazi wake.Mr Prezident chonde wonetsani mtima wachikondi chifukwa mawa nkucha ndinuyo ndithu.Zandale kumaziyika kutali paimfa tsatizani mwambo wathu wachi Malawi.Tinganene kuti kapena mukuopa kufa?kapena kutchona kwambiri ku America?Mr prezident kunena zowona ndinu wopusa kwambiri mbuzi mano kunsi

 60. But its really inhuman to hav such a type of a heart as a President.Even if we blame our own Edgar C Lungu, but he z a down to earth president compared to yo so called Peter.Wishing Chakuamba a peaceful rest of his soul.Mr APM, plz always remember the culture your beaultiful country has even if u stay in a small Lilongwe town.when u r in lilongwe, dnt think u re so special that u cant respect other pipo regardless of their criticism towards yo gvt.(thus if he criticised u at one point).My beloved Malawians, i am really mourning with u in this difficult tragidy of the loss of one of the Africa’s veteran politician.May His Soul Rest In Eternal Peace.

  1. Ifyo mulelanda ndomfwa nombafye nimbona ati bonsefye tamwakwanta intambi ishakukonka.nshakwata ifyakulanda pantu teinchende yandi yenu mwebene, mwaliishiba efyo mwikala.Bt dnt forget dat u wil also die one day.

  2. Yes he is but doesn’t mean he has no right to comments, our president is wrong papa Mr Stevie kaliati fufuzani history ya amene wamwalira Kaye sanali munthu wamba oti akanangotumako chabe nduna. He was suppose to present himserlf.

 61. Amene aja ndi a mtchona za ku Africa samazidziwa kwenikweni,anazolowera za kwa azungu,moti apapa sakuonapo vuto,teach him za chikhalidwe I mean you

 62. Ndale za Ku Malawi za ziii athu dzulo anayakhula kut Peter sapita Ku maliro angwanda atolakhani azodiac awapatsa headline ya khani zawo kusowa choyakhula, anakapanda president kusatenga nawo mbali yolamula kut malirowowa akhale mmNja mwa boma NDE munakatokota bwanji?

 63. How can the late visit a fellow late? Let’s think Malawians

 64. Abambo amenewa ali ndi vuto lopita kumaliro. mufufuze za maliro ambiri akhala akuchitika iwo samapezekako….. sikunyoza koma chilungamo and pachikhalidwe cha chimalawi timayenela kulilana…. inde sizokakamiza and si milandu koma kumakumbuka kuti nawenso utha kufeledwa and uzafuna athu okuthandiza kulira.

  1. Funso lako silabwino! koma nditha kukuyakha. Sindinapite. Sizingatheke malawi aliyense kupitako chifukwa zithu monga izi. Trasport. Matenda kutalikilana Komanso kusamuziwa yemwe wamwalirayo. Ine ndinakakhala ndi trasport yopita ku Nsanje ndinakapita kuchokela Ku Bt. ndipo amene anakwanisa ena amachokela ku Mzuzu and LL…. koma amene sanapitewa ndi muthu yemwe agwila naye tchito, kungolamula kuti ndikufuna ndipiteko zitha kuchitika osapisa nthumba lawo komanso ndikulandila ma alawance. take a good example of Dr Bakili Muluzi. Sindinawaone atajomba kumaliro a muthu wandale nzao or kwa athu ocheza nawo

  2. kkkkkkk ukuyankha ngati ndiwe wanzeru, iwe waku bt sukumudziwa gwanda? Iweyo unamva zoti president sakhala ndi vuto lomulepheretsa kupanga zina. Wanena bwino kuti mkosatheka wina ali yense kupita kumaliro pazifukwa, oky thats the point!

  3. Ulemu upite kwa Msogoleri wa dziko lino…. sitingamunyoze koma tingounikilana. Ndimakumbukila chaka chinachake agogo anga akazi anamwalira ndipo sanali oziwika or achipani…. koma chifukwa chakiti muthu wina amagwila tchito ku boma kunabwela a Yunus Musa and omwe ani nkazi wa Dr Bakili…… izi zinasonyeza kuzichepsa

  4. Mwina adakapita peter padakachitika chaxhilendo peter wa pulumutsa ndalama adakapita munali.inu nomwe kt waononga ndalama adakangotuma nduna,kd amalawi mwatani?kusowa zokamba eti?

  5. @ Fatima Bamusi Paja amati yemwe ali ku nyumba ya chisoni amapeza zabwino kuposa yemwe ali ku nyumba yachisangalaro. Kulilana ndikwabwino chifukwa moto umasata komwe kwasala tchile nde akuyenela kuziwa zimenezi. @ Joe ma “YES” bwana achuluka…. chithu chikalakwika sitikuyenela kunyoza koma kuzuzulana ndikuthandizana nzeru osamangoti Yes and enafe tikayakhula nde azitiona ngati ndife oukila

  6. Iyeyo ngati tsogoleri wa dziko anayenera ukaonekera kumwambowo … No matter what … Chifukwa anayeneraso kudziwa kufunika komwe gwanda anali nako padziko lino ndi ntchito yomwe adagwirako ….. Vuto lopeza zinthu zitakonzedwa kale limakhala limeneli anzawo adavutika kumenyera ufulu iwowo akungodutsa moyera ….. Ine ndili kuno Ku Durban sindikhathe kupita Ku nsanje koma nditamva kuti a president sanapite zinandikhudza kwambiri

 65. Pa chikhalidwe chathu amalawi apresident amayenera kupita kumaliro kodi akudikira kuti azamwalire ndani kut azapite kumaliro kapena akazawo
  .? Maliro ambendera sanapite apaso gwanda akazamwalira wachibale wawo ndipamene azanve kuwawa tonse titangotumiza ndalama ..the president must have humanity and put politics aside

  1. ngat analamula kt maliro ake akhale a chisilikali, is that nt enough? u cn c that but his attend? was there no one 4rm gvmnt?, dnt thnk childsh

 66. bye bye gwanda chakuwamba anthu mwapha aja muthawi ya akamuzu mwawapeza. ukatambatamba mkumayang’anako kumwamba. uthenga wanga mundipatsileko moni kwa akamuzuwo mukawapeza

  1. Jsephy Ramsey George ndiwe mwana khala chete phirikaniro ngati khutu la Njovu.Mvetsera amene ukuwanenewo anapha ndi Tembo 1983 mu May Gwanda aliku Ndende.Anamumanga chaka cha 1979 wamvera Mnyamata

  2. ayi che frzr kodi kukhala osewera mpila ndiye team yanu imatsewela ndi team ina team yanu mkuluza lnu. mulimomo inu tsimunaluze nawo. chimozimozi gwanda muthawi ya mcp bwanji amaleka kumaletsa. anzakewo kuti atsaphe n its not only gadama matenje ndiyambili so dnt say l was young l knew every thing muthawi ya mcp n now l hate everyone amene anali mu alamuliro wa mcp

  3. Mukamanena zakupha ulamuliro uli ose ndi wamagazi kumalawi,,,,,Dpp inapha Chasowa,,,anthu aja 20july 19 people kild,.Udf inapha Matafale,,,,ine ngat Mutumiki wa Mulungu musandiuze za ndale mumalawi muno Ma Prezident ali ndi mabulanda osati masewera.Nthawi ino si nthawi yochedwa ndi zandale,,,Mathews6 vs 33 tifune kaye Ufumu wake zose zizapasidwa kwa ife,,.Hosea 4vs 6 anthu anga akuonongeka kamba kakosaziwa.Accpt Jesus Christ as ur saviour,,,,,,,Amen.

 67. Pepani a Sena onse mtsogoleri wanu wapita koma mulungu akusankhirani mtsogoleri wina wamtundu wanu.Peter adzakufunani nthawi ya mavoti 2019,musadzalole kumpatsa mavoti anu mwamva!

 68. Miyezi yapitayo gwanda anaima pa nsonkhano wa dpp kunsanje,kuthokoza peter ndi boma lake pomuthandiza kuchipatala chakunja komwe anapita.komanso kuwauza anthu aku nsanje kut azavotere dpp ndi peter mu 2019,nde mwati peter sanapite kumaliro kwa mbuya?

 69. chasitsa zaye nchani kuti njovu ithyoke mnyanga? AGWANDA Dziko lanu lija la nkaka ndi uchi, lelo lasanduka la chiteze ndi sabola ,kkkkkk(amene ukudwa naye adza sanduka mdani wako) musathe mau

 70. Anthu inu ndakuonani ndinu owipa,munthu amadwala pompano sanachile bwino- bwino ayende mtunda onsewo.sizoona or muli inu simungakwanitse.

  1. aaaaaaaaaa!…Joseph choka amagwala nanga bwanji anakwanitsa kupita kukasegulira za ma nation I’d ls?

 71. tipatseni nkhani zotukula dziko lino ndi kusintha miyoyo y amalawi.osati (1)president sadapite ku maliro(2)kazako ndi phwake wa mbuya (3)dzanja la manja latupa(4)president akugonera mbali imodzi.mw 24 osatizelezeketsa

 72. Amenewa ndi anthu aja amatchuka ndi kuthandiza ndalama,chimanga,bokosi koma iwo samaoneka amati ndili busy kodi awo adzakhalanso busy?????

 73. I remember is whts john tembo said some years ago, that nanga kupita ku maliro amapasana ma invitation? Ndi ufulu wa muthu basi:D

 74. How could he attend the funeral yet he’s dead too. I had to read news for APM that he’s daed some days ago.

 75. Inuyo munapitako? Mzokakamizana Kodi? Peter akudwala, Peter wamwalira, Peter akugwilitsa ntchito mkono wamanzere,Peter wagula galimoto yondula lero..Peter sanapite kumaliro a Gwanda…Musiyeni Munthu pangani zanu zoti zikuthandizeni lol

  1. Dziko lonseli kumangokhalira kukamba za Mr President chifukwa chiyani??? Pangani zokuti zikuthandizeni mu umoyo wanu osati kuyang’ana zochita munthu wina ai mapeto ake tidzingotosanapo zala za ziiiiiiiiiiiiiii!!!!

  2. ndikumadabwa ndi a malawi magetsi avuta peter madzi peter agona ndi njala kwawo peter ndine mmalawi koma ndikukhala ku mozambique even here madzi,magetsi akuvuta kwambiri koma anthu anachi mvetsetsa sakupanga point peter go to zimbabwe ma civil servant sakulandira ma malipilo kulinso peter kumeneko?

  3. Wokuba yense mulungu amamulanga nde uyu mesa anabela mavoti dikilani mtundu umeneu umakomoka kukasala 2yrs nde Inu pheeeee tamulya nkhawe ku ndata kkkkkk

  4. Chilenje moti kukula kose zoona zingakhale zolemba walembozo? Usiyanise maiko watchulawo ndi Malawi , kwathu kuli ufulu oyakhula pomwe komwe ukunenako mwina ungoneneramo sunakhaleko or umangomva muma news ukanafusa Kaye.

  5. Audrey, iwe ungotenga point yomwe akutanthauza Chilenje kuti mavuto ali mmaiko ambiri.zomwe tikukumana nazo ife anzathunso akuziona.

  6. Peter anamupitisa ku hosp inu munapita kumaliro amene amamufunira zabwino ndindan pakat popititsa gwanda ku hosp ndikukaonamwambo wa maliro? muzitiso akuononga ndalama angoenda mmaliro?

  7. Eya Mr Kamoto gift koma koma sitingafananise ndi Zimbabwe coz kulibe ufulu president wawo ndi dictator, pano anagula magalimoto ambiri mbiri Ku Ministry of Internal security and Defence force pomwe other department sakulandilia like teaching, Ku Heathy, Chipatala chachikulu chaku Bulawayo komwe Mzimbambwe kwathu ko chimafanana ndi Queens 3 wks ago.anatseka coz kumasow zipangizo zopangira ma oparations, think about dat komaso akama panga zionesero kwa amene amangidwa akapita ku Police akumanamizira kuti no bail out komwe kuli akumawapha anthuwo.Nde osafanizira ndi Malawi we got freedom ngakhale abwanawo akumafuna kumasintha zinthu komabe we r better bra.

 76. to be a president of Malawi is a shame because u think like you are onthe same level with other presidents only knowing Malawi is the poorest but you wanna have the same treatment as the richest presidents. ..Gwanda fought for this independence. ..president was to go

 77. kukacha kukhalira kunyoza mntsogoleri wanu basi anakapita munakapezanso chonena , akuononga ndlama zaboma, ee alephera kumuthandiza alimoyo bwanji? I wud love ur CEO of Malawi 24 Mr L Chakwera wud advice u 4 silly post against APM .

 78. Peter yemweyo anatenga ndalama nkumuthandiza Gwanda kupita kuchipatala chachikulu ku India nde akanakhala ngat samamulabadira kukanatero,,,,, President akatanganidwa amatumiza nthumwi kumaliro komanso ntchito zina ziboma ndipo iziii sizinayambire pa Peter koma poti Malawi sachedwa kuiwala ndi ma blackout, kusowa kwantchito,kuvuta kwamadzi, kusowa mankhwala mzipatala kwatipezetsa chochita

  1. ndalamazo pitalayo anatenga za mtumba mwake?mesa anatenga za misonkho ya anthu.Ndalama zomwe anakaononga ku un zinali zamtumba mwake kapena zamisonkho ya amalawi?mumamutamanda pitalayo ngati alindithumba landalama bwanji?ndalama akukawa zaife tomwe apa

 79. Kumulhakho Kupita,kma Ku Maliro Achakwamba Osapita.Izi Zikuonetseratu Kuti APM Sagwirizana Ndi Anthu Omwe Anavutikira Malawi,amangofuna Kuwagwiritsa Ntchito Basi.Ndidali Komweko Ndipo Zinandikhudza Nditaona Bakili Akuyenda Movutika Pokaika Nkhata But Chinamkomera Kubwera Pamaliro,why Not Bwana President?Chonsecho Mbuya Wamwalira Ali Mbali Yanu,mukangofuna Kumu User Pansonkhano Waku Nchalo Uja Eti?

  1. Iwe ulinawo umboni, oti ma advisor ake amamuudza nzeru zopusa. Munthu ukukha chisa pogonanso nyerere zokhazokha, ndiye ukalankhule nkhani zakuchipinda koti iwe sulowako.

  1. kkkkkkk stupidity at its best! Dont you know dat he z a head of a state-in shot a father of a nation! You better go back to school bro!

  2. That’s the problem of ushering into power town mongers; 30yrs in diaspora & you expect them to respect our core values. The same president was also faulted for not attending Mbendera’s funeral. Despite that Gwanda’s funeral had military honour as per instructed by the state president, Malawians of sound integrity still strongly feel that it was of utmost importance for the president to attend this funeral despite his busy schedule as it is usually alleged.

 80. Mapazi anu.mumafuna akatani? sanatumize nthumwi oimira chipani? mumafuna akapepese ndizambiri? Zankutu! Komaso maliro samakakamizana upitako! Ngati palakwika nanu muzabweze, musazapiteko! 4tsek!

  1. Tennis iwe nde ndi mbuzi ndithu ulibe nzeru… Gwanda ndi munthu wamkulu pandare and he has political record than muthalika ..president ameneyu sayenda mumaliro nayeso maliro ake tizatumiza ndalama

  2. Zako ngati ndiwe wachitundu! Mumafuna adzatani? sanatumize nthumwi? Nkhumba yachabechabe usandisokose! Mxiiiiiiiiiiiiiiiii

  3. Komaso zoti kukachitika maliro muzikhala ndi list kuti akuti-akuti abwere pa maliro amenewa zithe! Do you think President sanachitepo kanthu pa matenda a Gwanda? Let him RIP.Tisaonanepo ma mistake.

  4. #hendrex sindikudziwa kuti ungakhale gulu liti la anthu, maliro ndi maliro basi,mukati wamkulu pandale ndiye kuti chiyani?

 81. pali ndi maliro ake omwe iye sangapite, monga nditafa ine koma kwa anthu ngati amenewa he suppose to go. shame on you mr president.

 82. Veteran nde kut chan? Zopusa ettt, amakakamizana kupita ku liro? Just coz he z the president? Inu mbuzi za mw24 munapita nonse? #shattap zanu

  1. NDE u mean dziko lonseli tisiye zomwe timapanga ulendo Ku nsanje?? Kodi gwanda ameneu ndi uja bakili amkati anamenya makofi Ku Mzuzu uja?? Coz ndaiwala

  2. Zitsilu inu d U think Pitala wnuyo ndiolungama.Chakwamba anathandiza ufulu wa amalawi.Pitala anapangapo chani, noonse hu r suportng his absence. Zitsilu…..

  3. Iyeyo ngati president ayenela kuonesa chitsazo chabwino chopita kumaliro paja iyeyo siwandale anangolowa ndi mutu chifukwa cha achimwene ok palibe kanthu

  4. APM analakwa chani? Anamutumiza ku India. Wamupatsa state funeral Gwandayo anali wa chipanii chanji poti he has been a rolling stone. Mmaliro sapita onse. konse anakhalako mumati apite ku maliro kenako muzikati chani.

  5. Symon phiri & ntumbuka, kwanu kunayamba kwafa munthu koma? Ngat muti eeeee, kunabwera presdent ngat? Ma zoba, as a prezdent, can just deligate others to attend that funeral.Mmafuna akapita mzit akuononga ndalama za boma? Hahhhhh! Womwalira sapita kumalironso kma

  6. Pachalo auze bro Peter aku dyelera ufulu oti anavutikila anthu ake ndiomwewo achina Chakwamba, Chihana ndi achina Bakili muluzi. Nthawi yomwe anzawo akuvutika Iwo amakabisala kunja ndi brother wake. Nde kusapita chikuoneselatu kuti ndimunthu osalabadira za munthu coz kungoonekela kokhako unali ULEMU wapadera ndithu.

  7. this is just stupid because late chakuamba was peaceful politician so we cannot express sorry by blaming one another for failling to attend the burrial of his remains.let’s unite to express our sorrow towards this painful incident.the president has done alot,lets thank him rather blaming him.some of you really attended the ceremony but during the whole he was in hospital you didn’t even contributed anything for his medication.you are just good at talking no sense.

 83. The other difference between this mthalika and the late bingu is awa amawonetselatu kuti ndi atsankho popanga zinthu….every year amakhala nawo ma function a mhlakho WA alomwe koma zikhalidwe zinazi sapitako and sanapiteko

  1. ndiyeno ngati anali pachibale zikugwirizana? iweyo ndi azibale ako aja mumachita zofana?, munya “, mesa paja mumati wafa , ai koma wabwera ndi mkono umodzi now ur talkng rubbish #LeavemrPresdnt alone useless pipo

  2. Tinyaadi sitikukana, but being the father of ths nation samayenela kumakhala ndi tsankho, he cud hav atleast attending other functions in the country not only organised by the Lhomwes, Now if the president chooses to celebrate with lhomwes then who shal celebrate with yaos, ngondes, chewas, tumbukas? he is a servant to all, not only one tribe!

  3. A christabel umbuli ukuwavuta kaya wayamba ma period mwina or mawuka akuvuta chifukwa cha uhule umapanga kuma tea esate Ku thyolo kwa mafisi…shupiti

  4. Nanu check omega bema mwalemba apazi its clear indication kut medulla oblingata wako nsempha umodxi sukugwira nthito, how came the whole munthu as ur kumabweka zopanda nzeru ngat zimenezi. apad ndakhulupilila kut ndiwe mphongo poti umavala buluku koma nzeru zako zili ngat za mkhumba

Comments are closed.