No more easy pass for Malawians to South Africa

Advertisement
Beitbridge

Malawians and other nationalities travelling to South Africa without proper documents will soon face tough times as authorities are planning to intensify guarding their borders.

According to the South African authorities, this is in line with the country’s crackdown on human trafficking rings.

The South African immigration officials have since identified Limpopo as a hot spot for syndicates involved in human trafficking.

Beitbridge
No more easy entry into RSA.

They said in Limpopo alone 77 cases were reported in the space of a week. The authorities added that 14 people have been convicted of human trafficking over the last two years while five cases involving the smuggling of people are before courts in the country.

An organisation called International Organisation for Migration (IOM) has been running programmes to raise awareness around the issue. IOM’s Zoe Rohde has disclosed that regional task teams have been set up to deal with trafficking in the area.

“And within those task teams there’s rapid response task teams which are the law enforcement agencies that actually tackle the cases and the prosecutions,” said Rohde.

He added that they meet on a regular basis and when cases come up they meet to discuss how to investigate them.

Advertisement

197 Comments

  1. Mukatilemba nthito mumatpasa k23,000 pamwez mkumat mwayesesa uko akupeleka R1500 pawk mwk and k 75,000 tangopangan maxamu kid pobwelela Ku mW munthu angakhale chmodzmodz akatdyetda ndiamanu? Alaaa

  2. Unnecessary comments ngati mukufuna anthu akhale akapolo aziko ndiye kazinyelani manyiwo inu mukudya nwino azanu akuvutika ndiye kuti ayese kumpusha ngini milandu asiyeni azibwela anthu akufika kuno opanda ma passport. Ndiye chowawuzila a home affairs a RSA ndizichiyani zausilu eti (masipa ako mfethu)

  3. Uku timati buu shit cause u dnt knw wat u talk abt tangomuwuze dat angoononga nthawi cause we have many ways dat we can pass to go there in RSA if u full up with amabojisi just keep yo mlomo close u must fuck knw dat mny fuck boses here he lv as make sure dnt fuck to take down again this masimba OK?

  4. When was it easy for Malawians to pass,I ve used this border several times,its always tough if u r short of documents…any boarder isn’t easy if right documentation r not produced…not worth printing Mr admin

  5. ndiñutso opanda zelu muķudanà ndiañthu añu pupita kunja kokadzisaķa tangoonani ñgakhale dziko lamalawi mmeñe likuonekela panopa khani yamanyumba zilibwino kwàmbili palibetu akumanga nyumba kumpotsa woyenda south Africa iñu mukhalila yomweyo yadzitupatu panopa eishi ndimbili yakale malo mosisa kuti achuluke otukula ziko mukukwezatsa mudula nokha ife açhinyàmata eeeeeeeeeeñdiye mwatilephela basi timayendatu waya waya malawi to south afriça ño chitupà iñu mukhalila yomweyo achitsilu

  6. amalemba iziyu mkut Ali mturo atagona mkut asanadzukei olo anasuta cha khotakota chochita kuphwanyaa Ndi mwala chija chifukwa ngati akufuna kut tisamapite ku joz angotseeka immigration asiye kupanga ma passport tiwone ngat mimba zawozo siziphwai mexa akudyera momwemu kumangokweza mitengo ya passport wik Ndi wik ndicholinga chomangofuna kutibera basi

  7. Ndudutsa border yapa Dedza nthawi imeyo magetsi atazima,anthu amene amagwiri ntchito amvere mdutsani ma computer lero sakugwira ntchito

  8. South Africa is where our ancestors came from the nguni ppo.so hu .ca stop us going back where we came from! U shit ppo I am sure u don’t know our history go back or history books and learn .we’ll b here until God come .

  9. amwene inu munali Ku USA kukagula expensive car ili LEXUS nde mukufuna kukhomelera ife tili kuno RSA kuti nafe tizaguleko ma 1series BMW #zalakwikwa pamenepa? inu zipangani zanu kumeneko nafeso tiyesese pangonopangono wonyengelera moyo wu MAN

  10. Evn if u can build a long electicified tower,putting heavy armed people & watsoeve, We WILL NOT STOP GOING TO S/A bcoz its where our lives situations atleast CHANGE.U SO CALLED govt have failled us,evn cant provide jobs for Us so MUMAFUNA KUTI TIZINGOTUWA POMWE INU ZANU ZILI BWINO? Tizipita ku Joni ngakhale mungapange bwanji

  11. That wont help!!!!If you go to the Lebombo border their is no border any more.They travell abroad as they like with no papers at all.Get the Defence force to do their dutys maybe then maybe it will work.Get rid of the CORRUPT OFFICIALS AT KOMATIPOORT AND THINGS WILL START CHANGING.

  12. anthu akupita kuchoka kuno ku Mzimba kupita ku John koma opanda passport nanunso mmadyera momo:dzulo ndikunena pano kamnyamata ka 12yrs kapitaso ku Rsa.kaya mmaboder mkumatani kaya….Mkunena za childtrafficking koma nokha mkumaloleza kuti ana ochepa adzipita:osatiuza zochita izo nzanu.

  13. kupusa basi,bwanji osalimbana ndi pitala wagula galimotoyo ma million ambilimbili malo mothandiza a malawi amene akuvutika ndi njala,magetsi komanso kugwetsa mphamvu ya kwacha kukhala yopanda value, timabwela kuno ndi ndalama zathu osati zochokela kwa amanu,muyese dala muwonanso munyela masipa.

  14. Kodi akulu akulu wa zamba zikuwapengesa eti osangovula kuti mitima itilibe ife bwanji kuti muli cha zombamu moti mufufuze njira yokhoza Malawi akhala wabwino kuti anthu asamapite ku mayiko kwina ayi? Kumangokamba za ziiii basi zamba zimakuphwetekani eti?

  15. tizivutika then u must Joke with us kut tizidya zitete ndi Mbewa..busy having sleepless nights thinking about bloking the way to South Africa aftr u cum up wth that fu*k u call yoself agenius..you hve done agreat Job…leaving behind your financial crisis around u…Mudzafa imfa yowawa

  16. Asiyeni apite kumeneko coz here in Malawi we don’t have anything to do and no matter what unagela boo but about working and money is very poor so we need to try which country is best so plz asiyeni achinyamata apite coz umphawi watikwana ife and tikufuna kuona kusintha

  17. Hahahahiest hahahah or nditi kikikikiest kikiki kodi mulandu owopsa ndi uti opanda traveling documents kapena kupha albino malawi24 mukadali mtulobe chifukwa chake kamuzu anali ndi slogan yoti kwaaaacha. Tulo kwambiri

  18. Kwawomwe mukufuna kubwela kuno musaophsesede kungo ika zonse manja mwa mlungu chilichose ndichotheka basi mulungu adalise onse ali paulendo wobwela ku JOZ KUNO ndipo alange onse opangitsa kuti mapasport akhale odula sharp!

  19. That’s bull sheet coz there’s no need to talk more about that while de country there is facing so much problems about poverty. Money belongs to the government only.sheet.

  20. Mukakamiraso kwambiri anthu Ali Ku SA muzaluza mavoti mosavutika kamba ka sanje akangoti onse abwerera sazavotera agalu inu a DPP foseki mbava

  21. u dnt know nothing cause uhavnt even clossed th boarder post,we wont gv up no matter wht tizbwera kuzaona anthu nkumabweleranso,who u.

  22. There is a serious reason why South Africa has withdrawn itself from the ICC. It is planning to become Africa’s richest nation once more. So it is planning to deal with illegal immigrants, by taking jobs from them and give them to its citizens. Open your eyes and see if you follow world politics

    1. South Africa doesn’t give jobs most jobs are from Foriegners to Foriegners,few are those that work for South Africans.

    2. We all know that foreigners are not loved by black South Africans mainly because according to them, they take their jobs and women. I remember in the last year’s Xenophobic attacks, the president (Zuma) said that people and the world must not blame south africans for the killings of foreigners. Which to me seems like he was allowing the attacks. We all know that South Africa is not a friend of the US but Russia while US and Russia are bitter enemies. So Zuma is taking Putin’s (Russian president) policies of running the nation. To them, foreigners are a threat, they weaken the nation’s economic growth. They don’t keep money in the banks (Indians and Pakistanis). That is also another reason why SA wants to allow only those with proper documents.

  23. Money is talking now ngakhale mutati ma solder anu azikakhala muma border nothing will change ife timadula or ndi pass yomwe ndilibe Juno Ku joni

  24. Kkkkkkkkkkkk mwandisekesa kowo,wowopsya usikuwatha omwewu anyamata akwathu okwana 15 atipeza kuno ku Pritoria 10 opanda ma Passport ndipo sikuyamba timangoyambilatu maplan pa Dedza Bodar kuzalowa pa Kalomwe ullendo kufika Chamano kuthananazo kutele tili Nyamapanda uwoo ! Zim kungofika Zim side basi timati tathananazo kuchokaapo RSA side BET BRAEGE basitu zikatelo kungofika MUSSINA kkkkkk kwayife satikwanisa kaya enawo osatiife akwa T/A kasumbu KU DEDZA AYYAAH

  25. U can’t stop some1 who z goin 2 abroad 4 searchn green pasture coz of document Never! koma ine kuno ndie kumandikwanila.

  26. MUNTHUSO OTHAWA NKHONDO AMAKHALA NDI PROPER DOCOMENT? AGALU ACHABE CHABE MUKUNGOONA NGATI DZIKO LIKUYENDA BWINO?? STUPID ZANU.

  27. Zopanda ntchito zimenezo, mutakhala kuti kapena pa borderpo mukaimika agalu kapena ndi kananena kuti zitheka. Koma munthu oti akufuna nayenso ayendere Benz panseupo, zimenezo ndizosatheka zizatentha miyezi iwiri yoyambayo kenako okha ayamba kuzipatsa transfer kuchokapo atalemerano.

  28. go to hell ine ndkubwela kumeneko posachedwepa ndkadutsa pomwepo komanso kubwelelanso komweko either kuchosetsa masiku mwachinyengo kapena kujampa kkk iwe ukungochedwa pamenepo buluzi iwe

  29. Zaziii. Chhomwe mungadziwe chinyengo sichizatha padziko pano. Muwakakamira bwanji anthu pomwe mukulephera kuwapatsa zotsowa zawo, munthu kumaliza xool ganyu osaipeza, aaaa anthu akuthawa ku gahena kuno.

  30. you are not solving the problems but corruption will be high as peoples would want to find ways of going to green pastes,

  31. Or atakhazikitsa #Chitetezo chokhwima anthu adzidutsabe bas coz nawonso achitetezowo masiku ano akufuna #Ndalama. Inu mukuonangati onse akupita ku #SA alindima #Documents oyenera? nanga mukuonangati amadutsa bwanji? mesa amangopereka ndalama bas, ziphuphu sizidzatha mpaka kale ichonde muchidziwe

  32. A MALAWI INEYO NDILI NDIKHUMBO LOZAKHALA MTSOGOLELI (PRESIDENT) WADZIKO LA MALAWI ,nkhalambazi zikuyendasa dziko mosalabadira a CHINYAMATAFE tili ku exile coz cha iwowa Ndilinazo njira zopasa achinyamata busy ndi ntchito ,ma business, ndizambiri ,

    1. Malawians ain’t hard workers but they have no option,so you do whatever you are given to save yourself,when you have no option you are saved from pride and accept the little you get for doing a heavy job,on the other hand South Africans refuse to work for little because they have the option where by its thier country.

  33. vuto nd lot saziwa zomwe akulemba pot anabadwila mmuno mu Malawi and akulanso nd moyo wa nsanje!!!!!Mwana wa ng’ona sakulira dzwe limodz!!!!Boses in RSA loves Mwians bt its Mw24 hate them!!!!Muzayalukatu nokha nd kaduka wanuyo

  34. Asaa!Mavuto Ake Amenewa Tikhalebe Ku Malawi Kuno?Tikupita Basi Nafe Tikagule Ma Android Ma Table. Ndidzayenda Pa Sache/lichelo Osatinso Pa Bus Ayi .Asaa Azikati Ndiyaonese Ndalama? Masiku Ano Tikangosizina Basi Tafika Ku Johnz. 1 Second Tafika. Tikupita Opanda Passport Kumene. Kk Kumangwetu Mangochi,makanjira.

  35. Kkkkkkkkk money talk. We always face tough time but where are we now? Tangoonani zauthimatima kwa magesi uko tisiyeni ife oyenda. We got our own ways

  36. osamachita post nkhani zachamba zanuzo mukakhuta mmakomomu musamatinyase ndi nkhani zofoira zanuzo enafe timakhala busy nde tisamaone zopusa zanuzi

  37. You are really true guys bcz, as we know here in S A . Without Malawians ndiyekuti Apolice akuno siziziayendera pa Beitbridge antu amadutsa pompo opanda paper lina lililonse. Komanso ama Taxi sizingayendenso, Azimayi apano pa Joni singayendenso Azungunso ambiri kuno amadalira amalawi omweo, So zonsezi zikugwila kamba ka amalawi ndiye zimene wapositazo sizingatheke pa Bettsbridge Lembaina nkani!!!!

    1. I object,looks like you just started traveling to South Africa,I remember 22 years ago before this crisis in Malawi,zimene mwachulazo zimayenda bho bho,pano nde chisimu tikuba amalawi.koma muziti a makonda amalawi chifukwa zilizontse “Yes Boss”, No objection even to salaries because of the mans condition.

  38. muzikauuza omwe alibe ndalamawo amene mukumawapeperesa kumudziko, ,,,,,,,,,,, zozweta zanuzo, ,,,,,,,,,no more, no,more chani iweyo document’s ulinayo olo uli kuwuukapoloko

  39. Zauchisiru zimenezo,akanayamba afufuza kaye chomwe akuthawira athu kumuziko.Akufuna tizikalima Fodya?zopusa akuguganizazo.

  40. Olo mukamanga mpanda ziko lonse tizaboola wautala jonz kkkkkk olo alondaanuwo tizawadyesela bwanji pamenepo

  41. Don’t worry admin anliponso ena anatiuzanso chimozimozi, koma chomwe wakonza mulungu chimatheka ambili omwe akupita kujon opanda mapepala ndiomwenso akutukula malawi

  42. Is there anything good in Malawi so that to bother ourselves to live? No! Only the lampat of corruption by the state leaders,poor educaton,poor roads,poor hospitals,poor food,poor electricity,no entertainment halls,no coverd stadium,no packing stations, 1 to 30 blackouts, we are doing our delopements by the helping hand fo God,what about just writting nosens things,we do eat nicely whatever want,we walk elsewhere want no problem God is with us,we shall be here till when we want to go back home. Nothing good in Malawi only wichcraft is their best thing they know to do

  43. Ngati pulezident akugula magalimoto odula. Osaganizila anthu ake akufa ndinjala. Kupanda nzeru kumalimbana ndi anthu othawa uphawi mbuzi inu. Simutikwanisa.

  44. Thank you very much, this is what I was waiting for.
    It will be easy to pass because they are launching corruption not though time.

  45. Yankho yazonse ndi ndalamatu basi anthu akumadutsa tsiku ndi tsiku.Even here in SA ndalamatu basi akutheka a Police kuwanikha ukudutsa mopanda vuto ina iliyonse

  46. Tatumiza nkhani ya ma coupon tilandila liti nanga ferteleza ayamba kufika liti ma admarc osati zachamba mukutumizazi ngati mulibe any post jst shut up ur mouth osati kumachita post zachambachamba zanuzi

  47. Iweyo ikumalemba izizi ifeyo tili nyatwa! Konkuno apolisi akunoku ndiomvetsa especially month end amatikhulupilira ifeyo amalawi

  48. Mukunadziwa mmene apolisi aku. South Africa amakondera ndalama simukanatumiza post yauchikapeyi kkkkkkkkk iwo amangoti make plan kuti udzipulumutse wekha ndie mukufuna kuti iwowo apolice akuyendyereni kuti akakuvera mukuletsa izi inu amalawi 24 muyambAna nawo amapolisa a southu Africa kkkkkkkkk ine kuvava kukoma in mzansi no passport pass free jst money talks ine ndilipheee stop this nonsense inu amalawi 24 mudzitumiza ma post okhudza fertelezer poti nthawi ino ndiyoona zakumunda osati zachambachamba zanuzi apa mwava

  49. Anthu samafuna kuyenda opanda ciphaso coyendela ai koma mmene cinadulil muja kodi angakwanitse ndi anthu angati? ulova,umphawi,ndi umene tilinaou koseku kumakhala kufunafuna ntendele kunena zoona kumalawi kuno akusangala ndi a nthu akunja achimwenye amene aphangila ntchito zose za ifeyo acinyamata ngati mwai ulipo kumapita basi kujon konko

  50. Aaaaaaaa ngan nimtereshede nganga vaziii lizdutsabe maborder mu nabola mtere pathumba baxiiiii #vuuuuuuuuuuuuuu pezan njla ina

  51. Iam the one who travelling to south Africa without proper documents i dnt have a passport nothing koma ndimayenda bho boo chithumwa chimagwira ntchito akamaona ine amaona nyerere mwamva? Why ndimayendera chithumwa cause passport yikudula kwambiri ukapita ku immigiration amakuuza kuti ya pompo pompo ndi Mk150,000 nde ndinaona kuti tikungowalemeretsa anthuwa…

  52. Malawi 24 ur fools i dnt think u fuken reporters u went to sxool .can u see whtever u hve been posting and see hw u hve been fools. Who is paying u stuped pple reporters? Or ur just coming in for the seek of ur abdomen.? Start writting abt peace u fools

  53. The more you talk the more they’re traveling without even proper documents just because they’re looking for green pasture.

  54. BOMA LAKHAZA KUNALI AMZANU PANO NDI AKABWELEBWELE AKU KHOTI,ANTHUWO AMAYENDELA NDALAMA ZANU?E!E!E!MUKUWAPUTA DALA AKUMANGOCHI MUYIZIWA (KUNUFAYAKUNU)

  55. Malawi wake magetsi akumangoyaka usiku okhaokha mkumati munthu uzipitilir kukhala kuno? kumatani? Ndi move yanji yotheka yomwe munthu ungapange kuno.. Ndikwabwino kukazunzik kwa eni. Boma chimanga kumadula kuposa chogulitsidwa ndianthu wamba. Atsitse zitupa kt anthufe tithawire komwe tikapeze mpumulo.

    1. 40% ya beget yaziko lathu timachitakuthandizidwa koma Malawi 24 amaonangati iwowo ndiwoyima paokha zoti nchimozi mozi ndiopepha mmiseu saona mkumanyoza osambisankhalamba kuno komaaaa mmatumbamwao mulii –00 kkkkk

    2. kikikikikikikikik. Bucket ya 5 litre yachimanga inali k1100. pano Boma latsekula ma Admac chimanga akugulits k250 per kg. #CHOLINGA akufuna kt osawukafe tife kapena kt malawi timuthawe? Ndikawaganizir abale athu kumudzi akwanits 13500 per 50 kg. Zachisoni kwambiri.

  56. Pasport ndindalama malo awa anthu ama opa aneba okha aja basi osati south africa makolo a frozy samava zoti anthu akungo dutsa

  57. Makape inu eti?? chimene a Malawi akuthawira kuno ndi chan? nanga mukuwakakamira ngat u can provide their basic needs bwanji? tonse achinyamata tikhale opempha bax?? #Tiyeni_tikakunana_ku_msewu_konko as late #Bingu said

Comments are closed.