Nomads to face Zolozolo F.C in Fisd Cup quarterfinals

174

Central region FISD challenge cup champions LAKE Valley found themselves outmatched as Yasin Osman’s side showed no lack of pace and attacking aggression at Civo stadium to reach into the quarter finals of the Fisd Challenge Cup.

Two goals from Peter Wadabwa and a goal each from Jabulani Linje, Mike Kaziputa, and Khumbo Ng’ambi were enough for Mighty Wanderers to book a date with Zolozolo United in the quarter finals of the Fisd challenge cup.

be-forward-wanderers

Nomads will face Zolozolo in the quarterfinals.

The match started on a higher note but it was the Nomads who showed no mercy from the word go as they were dominating possession and attacked in numbers.

Wadabwa opened the score line inside the opening 10 minutes of the first half after the Lake valley defence was caught napping in the line of duty.

A few minutes later Wadabwa was celebrating once again when he bagged the Nomads second goal of the match and the first half ended 2 nil in favour of the Nomads.

After the break the Nomads come in with fresh ideas as they kept on dominating the proceedings at Civo stadium and from that angle it looked that Mighty Be forward Wanderers will decorate their Fisd Challenge party with a riot.

Minutes after the recess Linje increased the Nomads lead when he bagged the Nomads third goal of the match to completely put the game beyond the reach of Abbas Makawa side.

Midway through the second half Kaziputa scored Nomads fourth before substitute Khumbo Ng’ambi completed the riot at Civo stadium in Lilongwe.

After the match Lake Valley coach Abbas Makawa conceded defeat whereas Nomads coach Yasin Titch Osman thanked his boys for the win.

Mighty Be forward Wanderers will meet Zolozolo fc in the quarter finals.

Share.

174 Comments

 1. Ine ndinamva makolo anga ndili wachichepere kuti, mwana waulemu pakhomo amadya zabwino kapena kutinso amapasidwa zabwino ndi makolo kkkkkkkkkkkkkkkkkkk mutanthauza nokha

 2. Noma ikungodusa moyela kkk pano Zolozolo Kkk.. the same thng was wth Carlsberg, thy played Mangochi Police, Prison United… mmm somthng fishy here.

 3. Nyadirani popeza commitee yanu ya Fam idzakhala pomwepo mpaka muyaya, koma tsiku lina muzaonekera poyera, adzikukonderani chocho, akungokupatsani timatimu tosadzika komwe,ndiye mukuyankhula motubwa ndikuzipopa, funsani malemu omwe mtundu wa malawi umati ndi wamuyaya ali kuti, masiku amathera kuchitseko tidzaona patsogolo pano

 4. Inu mmesa mmadzipopa? ndinu timu yafuko nde mukuti akupatsani akuluakulu??hehehe ndimmene muthele muzigwila tiyenazoni ndimatama anuwo,simumati simumagonja?? lero ana angokuvinitsani m’bwiza bac.kkkkk musova,!! ine ndikuchongelani.!!! 4waaaaaard.!!!!

 5. m`dani wako sakupuma bwino kkkkkkkkkk please osaganiza mwa umbuli iwe NEBA kkkkk zonsezi zikuchitika chifukwa cha draw yomwe palibe angasinthe••kaya iwe nditsoka lako potola siliver

 6. Koma yaa..! Zimenezi ndiye ziti? Presidential cup, Carlsberg cup lero ndi fisd cup.. Nyerere kukhala team yokhayo akuti yongotola Wandalazi youth, Prison utd, Mangochi police, Lake valley, Zolozolo, Dululu..! Weaker oponents? Izi mkumati Zampira? Mpakedi Nyerere kukhala #6/8 Super league! Kodi inu mukudzitcha atsogoleri a ma bungwe azampira ku Malawi kuteroku ndiye mmati kupititsa masewero a mpira wa miyendo patsogolo? Mukuthandidziratu kuchotsetsa ntchito ma coach ku Nyerere!

 7. Mapwala anu a noma nonse,winning against these little teams & ur proud of that??? Muzamenye a big team like silver then we gon knw u da best

 8. Abale anga musadabwe sizachilendo izi Nyamilandu amaikondela noma chifukwa ndi team yomwe ankasela nthawi yomwe ankamenya mpila ndiye chotsatila ndi chani kuikondela basi koma akunama bola ma banker’s atenge cup imeneyi cholinga Nyamilandu achite manyazi ine wa NBB.

 9. zodabwitsa izi kodi bwanji Noma amangoyipatsa tima team tingo’no tingo’no, iwe FAM , you must be very stupidy, shame on you, BB sizamenyaso cup coz kukondera kwa chuluka, Noma reserve fc, mangochi police, zomba prison united, tchewu boys, pano kumati Zolozolo ? Foolish

 10. 90 + Minutes kulephera kumenyera pagolo ati ku defender kudikira Mapenalty Zamanyazi bwanji,, Nde enanu mumati ” PENALTY FC ” Ndi The Peoples team Zitheretu ndipo ndisazamvesooooo

 11. Neba mutokota mutopa munamenyedwabe basi ndipo simunati mukana kwapulidwabe loko muligimo muzikwapulidwamoso muziona mwakula mwatha

 12. Akuziwa Kuti Noma Sitha Mpila Mchifukwa Chake Akumaipasa Tiwana, Nanga Lake Vally Mkachani Nde Mukawina Basi Meeee! Meeee! Ngati Mbuzi Mmastreetmu, Ikhale Team Yeniyeni Mukaichinye 5-0 Tizakuonani Ngati Mutazaduse Pasilver.

 13. Ndiye kuti pakati pa zolozolo ndi neba kulu ndi ndani? Neba iwe watulusidwamo pomwe zolozolo alimobe ndiye ukuti ndi mwana? Mutu wako sukugwiradi wapenga kkkkkkkkkkk. Ndiye sunday usamale akumenya ku nkhongo ubaizika ndithu.

 14. Ineyo ndikamamva kuti ayi noma amangoipatsa ma team ang’ono aaaaah ndimangoona kusautsata mpila kungozivera mu news paper, ngati simukuzitsata za mpilazi kungokhala, koma musaiwale noma pa ndalama kkkkk eeeeeh ndi nkhani zina kuteroko apanso kaya wina afune kaya asafune Fisd Challenge cup ikutenganso

 15. Let the losers talk, what ever they won’t, coz that’s our expectation. Therefore we thank God for helping us to move forward.

 16. Zimawawa chonchotu mukaluza iwe neba, komabe siunati nangasi akusinjanso mzakoyu sunday ikubwerayi kodi. Mwano iwe, Noma woyeee!!!

 17. Ukanena Za Noma Utopa,NOMA ILI PA CHIONGOLERO CHA FISD CUP, SIZIFUNA KUSUTA FODYA UTSI WAPEMELEDWA MMASO BLESSINGS TEMBO UMAITHA,KAMBA ZAKO NEBA

 18. Ndachipezano Chifukwa Chimene Osewera A Team Ya Noma Sachita Bwino Ku Flames.
  Nanga Imeneyi Ndi Fixture Yotani?
  Soccer Will Never Develop In Malawi..

 19. Mvula ikagwa kuchuluka zoliralira. Pakatipa bb yakhala ikupatsidwa ma penate odabwitsa koma otsatira bb samadzudzulapo.

 20. kkkkkk tingopatsidwa mitsamiro yabulets yokhayokha koma beware wanderers paja a Zolozolo analonjedza kuti timu yawo ifika mpaka kumafinals mwina aponda mwala ngati mmene anayambira neba dzulo kuwadza mikodzo ya finye pagolo la Silver kkkkk mikodzo yafinye munaitenga kuti?

 21. siyani kuganiza mwaumbuli…..wen the draw was conducted,every team representatives was there and they all impressed with the outcome….NDE muti fwe fwe chani…..
  #mukambirana simunatiiiii

 22. kkkkk Osalira mesa! mumati Team yanu ndiyayikulu ya Fuko La Asamunda ndiye akamakupasani magame Amakupasaniso! Okulilapo mzeru mumpira. koma vuto ndi nokha! mumalora kubandulidwa Chisawawa.

 23. At noma amaipatsa game ofewa nanga wizards fc ndiyolimbanso kkkk ukufuna chiyani nebe basi noma isamenye wa kampopi fc akumane ndi zolozolo fc guys zikhala bho eti?. OSAIWA KUSUTA KUMAWONONGA MOYO. The wise people’s choice{NOMA} Eee

 24. ndichifukwa chake mu league mumangojowamojowamo chifukwa mulibe size yanu,inu ndinu ofunika muzimenya ndi achina zolozolo, lake valley,dululu,sayama ndi migowi

 25. Hahaha kodi mukuti Noma akumayipatsa ana inuyo nde kuti akumakupatsani matimu opitirira usinkhu wanu? Mpira ndi wozungulira uwu…mumpira mulibe ana…Bullets inavutika ndi Wizards mpaka ma penalty…Noma inadutsa mwa Wizards mosavuta…nde muziti mumpira muli ana? Limbikran tikumananso chaka cha mmawa…ziganyulan! #Noma

 26. This is why mpira pamalawi pano sutukuka, ziphuphu komanso chinyengo. Kungomva kuti technology inativuta pamalawi pano choncho mumangogwiritsa ntchito manual, ndiye basi zizingolowa chipwirikiti?

  • ine oikonda team yanga ya nyerere #B4_WANDERAS_MANOMA zimandiwawa tikamazikweza,kuzitukumula komanso kuzichemelera kuti team ili bwino tikamamenya ma team osachuka mma cup pomwe league tikuvutika nayo,chanzeru palibe kunyadila kuti tamenya #LAKE_VALLEY pano timenyenso ndi #ZOLO_ZOLO,ndimafuna team yanga #NOMA_AKA_NYERERE tizitibula ma team omwe alipamwamba pa #LOG_TABLE yathu,
   ……mosaopa man mpira ndimautsata monga inenso player wotindamenyapo mpira team kuti ichite bwino izimenya ndima team olimba muziko,ndiye ine oudziwa mpira palibe choti ndizinyadira akamatipatsa ana iyaaaa,
   ndingotinso #FAM_#_SULOM mbolo zanu zadwala chindoko komanso nyini zamanu zonunga mwamva,mkuonjezera kuononga team ndinu chifukwa tikaawina ana ma player amazimva akakumana ndima team odziwika kutibulidwa.

   INE ZIKUNDINYASA,ZIKUNDIWAWA KWAMBIRI MONGA PLAYER OZIWA MPIRA KOMANSO #NYERERE_SAPOTA_NUMBER_ONE.

%d bloggers like this: