Frozy takes Malawi by storm

Advertisement
frozy

No wonder that almost every Malawian is aware of this drink called Frozy. You can’t mention any place where you can escape the name Frozy when you are talking of soft drinks in the country.

In weddings, bridal showers, almost in all gatherings in the country, Frozy has been crowned a leader among all its all substitutes.

Malawi needs to make an analysis on why this Mozambican made fizzy drink has permanently planted its roots in the country.

frozy
Frozy; Has hit the market in Malawi.

Malawians we spoke to claimed that cheapness of Frozy compared to its alternatives has massively helped it to conquer the soft drink market without mercy.

According to Lilongwe residents, Frozy in the Malawi capital city is going at K200 which is cheaper compared to its substitutes.

One of Lilongwe Residents AbdulRasheed Asima told Malawi24 that the coming of Frozy has helped him to cut his lunch spending since with only K300 lunch is made possible.

“In the past I was spending more than K500 for lunch and according to my monthly salary that was overspending,” said Asima.

In some districts of the country like in Balaka, Malawi24 noticed that Frozy is being sold at K180 which is half price of its substitutes. In areas that are bordering Mozambique Frozy is going at K150.

Malawi24 has also found that the domination that Frozy has put on locally produced soft drinks may have negative impacts on the economy of the country.

Since market is determined by forces of demand and supply, the coming in of Frozy has dwindled demand for locally made alternatives.

This low demand is likely to force producers of these locally made soft drinks to reduce production percentage hence loss of jobs among Malawians may be experienced.

The Balance of Payment of the country may also register a deficit because money will be spent on importation of this product which is made outside the country.

Malawians indeed accepted Frozy as their main soft drink because of its cheapness but the imported drink will eventually affect the country’s economy.

Advertisement

272 Comments

 1. Anthu anyanyala fanta ku msokhano akuti akufuna Frozy. Akuti’ asaaa ife sitimwa fanta antaa, timatomwa frozy kamba khakuti fanta amatokhalamo ochepa komaso amatoumila sugar. Frozy anatoikhamo wa phulayizi 50 (meaning frozy is 350 mls and fanta is 300 mls). Khomaso awa amaphika fanta wa amatotizunza nao mabotolo awo ati tibweze maziwo akhathamo. Frozy amatotipatsa ndi botolo lomwe tinkhe nalo kunyumba natiguliramo mafuta ophikira. kkkkkkk So you can imagine this being said in Lhomwe accent.

 2. Are you good in bed ?Do you really need a rich sexy sugar mummy or sugar daddy that can change your life completely with money and influence, so get the opportunity to meet sugar mummies from all works of life,politician,bankers,oil ladies,executives,directors,gold ladies,cash money ladies,Global Network group friends,doctors, ladies, willing to pay as much and get the best exclusive VIP arrangement anywhere in Nigeria,LAGOS,ABUJA,CALABAR,DELTA,ANAMBRA,PORTHARCOURT,,RIVERS,KOGI,KADUNA,JOS,ABIA,KANO,BAUCHI, SOKOTO,BAYELSA,ONDO,OSUN,OGUN,BENIN,IBADAN,ONDO,BENIN, call admin on 09036713792 08117333727 for your connection,like page before calling.

 3. Frozzy ndi deal, I like uja wa Green ndi uja wa wokhala ngati Sprite, once I buy this drink personally I see 67% difference to our usual Fanta, Coco, Sprite, etc made by Southern Bottlers, this drink is also flexible in terms of pricing and tasty too. Frozzy ndi dhilu koma. In Tanzania there also many types of drinks and Fanta or coco is number 120 away from other beverage, here in Malawi since we had no chance to choose other types of beverages fanta and cove rose from normal prices of K50 to K250-K400 killing all poor customer’s wish to quench their throat with a soft drink, now Frozzy is an answer to all of us.

 4. Frozy akuyenenera kuletsedwa kulowa mdziko muno. Do you know the Effects of those frozy bottles this nation, Zizationongera chilengedwe and cost yobwezelesera zoonongekazo izakhara yambiri than K200 mukuti ikutchipayo

 5. Hahaaaa awona kuti anthu ayamba kutsiya kugula ziachina fanta, coke zimenezi, business ya ma soft drink yasika kuyenda nde mwati tiwanamidze a Malawi kuti frozzy chani chani, sitisiyabeeee kumwa frozzy mpakana kalekale, mwakuma ndi competition ndi frozzy mumayenda mbaliii

 6. ndikuganiza kuti ambiri mukuika ma coment ndinu anthu okonda mpira ndiye frozy mukanasiyira ine chifukwa sindikonda mpira 1 qustion kodi chikho cha carsburg chipitirila ngati inu okonda mpira mukugura ndikumwa flozy muganize booo simukhauritsa sobo company koma mudziranga nokha kkkkkkkkkaya,.

 7. ndiye mwati mbewa zina zikuretsa flozy? mukumbukire kuti m’dziko mukakhara chakumwa kapena chakudya chodarilika chimodzi kampani yopanga zimenezoyo imakhara yotunphwa fanta 300ml k300 flozy 350ml k200 kuribe flozy wambora sobo company isanapangepo chakumwa chokoma ngati flozy l love flozy

 8. Its not good for children it has too much acid, thats why its cheaper than coca-cola fanta & sprite. Taste Frozy and tast fanta or coca -cola notice the difference. Osamayamikila zilizonse yambani mwasiyanitsa ndi ndizakelezi.

 9. these companies will buy them off if they see Frizzy is making money and people likes it.Maza was originally from India but Coca-Cola bought the company off because they saw people liked Maza.by the way where is Tobwa poti ndi deal,cheap,traditionally tAsty and sometimes I wonder zathila …….

 10. A!!i ine kudabwa masacheti chani ngati amazikana aniake inu bwanji kwenikweni tiyenaloni basi lama k50 li thobwa basi less acid more erngey no effect much diet

 11. Or Mutandiyika Doom Mkamwa Ndizimwabe Fronzeyo. Ndimageba Ndekha Kut Ndipeze K200. Iweyo Ngat Uli Nazo Zocholuka Zimwa Zodulazo.

 12. chomwe chandiseketsa ndichakuti a Malawi24 mwayika ma empty bottles kusonyeza kuti mukumwanawo frozy… Tikhoza kumagula zakumwa zopangidwa kumalawi komkuno koma vuto zimadula china ndichakuti mabwananuso tikakulemeletsani mumatitenga ngati ndife zitsilu nde bola frozy yemweyo coz akutukula anthu ama-business ang’onoang’ono zoti kaya akuchoka kuti ndilibe nazo ntchito

 13. Frozzy frozzy frozzy…how many times have i called you? heheee continue your job kuwamvetsa azokumwa enawa kuwawa… tidzakumwa mpakana Yesu kubwera asafuna asiye apo biii alira basi…with or without acid heheee odi ukoooooo

 14. SOBO ikudulitsa zakumwa zawo ,komanso anthu akumalawi sangaziwe kuipa kogula zithu zakunja choncho tangoyetsetsani kutsitsako mitengo ya zinthu zanuzo

 15. Inu inu amene mumakoza frozy mukusokoneza malonda asobo azanu coco ndi k250 + dipost k50=k300 inu k250 no dipozt chibotoloso chachikulu musamale2 south a many it’s an I bwanji bwanji mutamamenyako kadipozt kawez katuwentey ba kokha kabotoloso kukajudula kakhale small kenakake ndiye kut pamalawi pano mukhala kkkkkkkkk kupanda kutelo eeeeeee mbola

 16. We are paying tax almost everytime we place our hand in the pocket. Everything is taxable. We are trying to save monies here zotchipa zabwino zapezeka ndisagule in the name of kutukula dziko olemera azilemerera ife osauka kumangosaukabe boma pezani njira zina zopezera ndalama nkhani isakhalire msonkho penzani nzeru zina. Zimandinyasa mukamadandaula za misonkho. Try to find other means of generating income. Ndalama zomwezi za msonkho anthu anatibera cashgate. Msonkho wa anthu ovutika unalowa mthumba la zikhwaya. Lero I want to make good use of my hard earned income you come talking shit dont buy zotchipa sizabwino. Why mukutiramula do you give us money for free? Salaries are very low chiperekereni misonkho. Dont blame azungu ndalama tinaabera azungu thats why they pulled back their aid. I hate zotiramula ndi ndalama zathu aliyense ndi wamkulu more over Cocacola si company yathu go to hell

 17. welcome frozy,bola kulemelesa mocambique coz we know 4sure atigaila mages, osatawa akungokhutisa mimba zawowa ukauza blackout akumangeso,frozy ndi dilh

 18. Ine or kumugwira frozy ai ndipo sundingamwe mkomwe ai! Ine ndimamwa za quality za” sobo” mburinu zimwani zi ma frozy zanuzo ma drink ama Vendor ine ai konseko kufuna kugwetsa achina fanta akunama sobo iri pheee ikudziwa kuti ozindikira ozitsata atipeza.

  1. It’s supposed to be one of the most closely guarded trade secrets on Earth – so secret that only two employees know it at any one time. The recipe of Coca Cola contains a list of ‘secret’ ingredients known as ‘7X’ – herbal extracts which give the drink it’s unique flavour, which the company has guarded for a century.

 19. A SOUTHERNE BOTLES VOMELEZANI KUTI ANZANU ABWELA KUZATITHANDIZA MAKABUDULA ANU OTALIKA MALISANIWO AKHWEPA AMENEWO FROZY TAMULANDILA MWACHISANGALALO

 20. Just stop talking and make your products more beneficial to the consumer than that of the competitor people will buy. Malawians can not be cheated buy names you call the counter product just because you want to monopolize the market

 21. What you should know cocacola and fanta company are long stayed. Their drink has quality standards. Give them few years you will find frozy no where in town. Old bloom knows the corners of the house.

 22. A country like Malawi with 85% of its citizens illiterate is very difficult to understand the dynamics of the economy and its impacts

 23. All we are doing is making an unknown Mozambican company rich while our own will one day lay off it’s employees or shut off completely. Who wins then? But again it’s through corruption that this drink finds it’s way into Malawi, either by dishonest citizens or corrupt mra officials giving way. But again it’s none of my business anyways because corruption is from the head

 24. Mukunamatu inu timwa frozy ife.!! munatijaila kwambiri,kabotolo kakang’onong’ono 250 pomwe frozy 350ml K150 Kwathu kuno nde ndimmene ndalama zasowelamu basi muzitibela? alaa achamba inu eti.!! mwatilemelera kwakwana tatopa ndikumwa mabotolo osweka .frozy ndikamwa botolo ndimampatsa Tauraie chidzukulu changa kuti chizipangila zawana koma osamucheka.basi munazolowera kuika miyoyo yathu pangozi ndi zosweka zanuzo?? He he he he Odi ukooooo frozy adutseeeeee..!!

 25. Ndi Ziwanda Za Mphepo Izi Frozy Zisiyeni Ziduse. Mukudandaula Kuti A Southern Bottlers Amakumwesani Mabotolo Akale Mesa Paja Akuti Tizipanga Reuse,recycle Kuti Tisaononge Chilengedwe?Tsono Frozy Mabotolo Ake Mukudziwa Kuti Akuononga M’matauni Athu?

 26. Umbuli A Malawi Udzakupwetekesani. Mumatsata Zotchipa Kusiya Zomwe Zingapindule Moyo. Mchimodzimodzi Kugula Bonya Kusiya Madzila Pamene Madzila Ali Ndi Ma Vitamin Ambiri.Frozy Amene Mukunenayo Mukumakhala Acid Wambiri Amene Akuyambitsa Unyang’anya Koma Zikumatenga Nthawi Ndithu Kuti Munthu Adwale. Kumaganiza Penapake Simungatukule Dziko La Kwina Kwanu Kuli Mavuto.Cocacola Ndi Fanta Ndi Zina Zotero Ndiye Zakumwa Zakumwa Zabwino. Zinazi Muzizisiya Ziduse Ndi Ziwanda.

 27. and mukazakonza magetsi kumalawikuno kampani ya frozy izabwela konkuno and tizigula k70 mmodzi ! kuzabwelanso kampani yotchedwa kingsley and zakumwa zizatchipa heavy , koma break yemwe akumanga zonsezi ndi magetsi BASI

 28. This is not our own product. I am not sure if our govt is getting anything from frozzy sales. A Malawi timajijirika ndi zili zonse. Ukamwa Frozzy, amadziwa ndi mwana yemwe, kupenta lilime. MALAWI GOVT, MBS & SOBO GET THIS DRINK OUT.

  1. 1:Ngati ulinazo ndalama usamaganize kt aliyese alinazo azakofe tinabweleka ya air time ndiyetikagulenso zodula……. 2:ukuwononga chikhalidwe cha amalawi chosatukulana tokhatokha…

  2. Ada Kumwenda, kugula frozy sikuti ukutukula mmalawi nzako ayi. By and by tidzava kuti SO BO atseka anzathu awachotsa ntchito. Ndilibe ndalama ngati mmene ukuganiziramo koma makampani athu ena akupanga zokumwa ngati zomwezo. Lets give them enough support. Frozzy waononga misika chonsecho siwakuno.

  3. Sory guyz chichokeleni kumeneko ndi kale,kodi frozy yo pokumwa amamveka ngat coke,sobo,juice,kapena chani? Plz let me know coz mmene ndimachoka kumeneko mkut kulibe such type of drink

  4. Semu, Fanta ndi Fanta, Frozzy sakufikapo and wangochuka chifukwa choti ndichakumwa chatsopano, chotchipa komaso sumabweza botolo. I tried it one day, aaaa choncho chakonda nzako mlekere.

  5. Semu Ofatsa, You are right. One day I went to buy a bottle of SOBO squash and ended up buying a new Malawian product called Choice Orange Squash by Choice Products Limited of Luwinga, Mzuzu. It is as good as the original sobo squash. We better go for such products.

  6. Kmadi guys frozy yo siwakumalawi ndiwa mozambiq chomwe mungadziwe mukutukula mozambiqyo kmso fanta ndi fanta makomedwe ake sizingafananendi frozy

  7. Kmadi guys frozy yo siwakumalawi ndiwa mozambiq chomwe mungadziwe mukutukula mozambiqyo kmso fanta ndi fanta makomedwe ake sizingafananendi frozy tatiyeni tilikonde dziko lanthu amalawi

 29. Kmano a malawi beaureu of standard mwayeza kt mulibe vuto lina lililonse mmenemu kt kutsogoloku xidxatibweretsera ma problem?ngati chonde muwerenge uthengau chonde ndiyankheni chonde chonde ndagwira mutu wanu kkk fukwa tisamangokondwera ndichifukwa tikungodwala matenda ovuta maina

 30. Dziko la Mozambique ndilodabwa komanso kukhudzika kamba ka mankhwala otsukila mmutu omwe company ina kumeneko imapanga.. mankhwalawa ati amadayila tsitsi koma ku Malawi anthu asandutda zakumwa zozizilitsa kukhosi kkkkk choncho boma lat aliyense apezeke akumwa azengedwa mlandu ofuna kuzipha ..

 31. TImwe zimenezi basi nanga enawa aziti mabotolo ngopelewela ndichifukwa chake zokumwa zikusowa ntengo mpaka k300 kabotolo kang’onong’ono frozy ndi dihlu makamaka wa uja wa Black.

 32. Frozy Ndi Dhilu,k150 Kumwa,Botoloso Kutenga…K100 Kugula Obama Pamene Cocacola K250 Enanso K300 Imene,Mubafutsa Kkkkkk! Maukwati Frozy Wadyaso Wani…

 33. Frozy is not a good drink healthwise.It contains a lot of acid.By buying frozy it means you are promoting Mozambiquean company to be rich and Malawian companies to be poor.In the end the same people who are appreciating about frozy will be retrenched due to the poor sales by the company.Why do Malawians like cheap things? Umphawi uwu utipweteketsa.

  1. People thought that when you are poor and uneducated it means you can not think rationally but the opposite it’s true. The poor are speaking with there actions. Substitute effect due to price increase.

 34. kodi mvuto kweni kweni ku company ya sobo ndi chani?.your soft drinks are very expensive y?.cant u see kuti even your quench water is bein droped on the market becoz it is expensive?. u need to upgrade your standards of makin your drinks otherwise u may loose customers.cant you make a rid of a bottle that can be easy to open without using involving someone who has an opener to open for a customer?.customers feel good and protected wen they open themselves the drink they want to drink.muli ndi zaka zingat mukupanga zakumwa kut mpaka pano u fail to make nonreturnable bottles?.mabotolo omwe azigogo athu anaika milomo yawo ife tizimwela omwewo?.kkkkkkkk.tizimwa zakunjazi basi.

 35. Don’t bring lies here. Who has proof that frozy is being smuggled into the country from mozambique? Zolowa muno movomelezeka izi

 36. Where is MBS,MRA….. do we know the effects of this drink apart from being cheap?! Do Malawians know that by smuggling this product into the country we are killing local industries that employ fellow Malawians?.

  1. Popha nyani sitiyangana nkhope. We are paying tax on everything you can name it. School materials to water. Buying this drink will save us some little cash.

  2. It seems it’s our long time culture of not caring our lives! How many do observe even expiry date when buying? Frozy has no expiry date !

  3. But do you know that it has high acid content? And that people are also using it to clean toilets because of this and it cleans toilets to sparkle? Ndiye what more m’mimba mungakhale bwanji?

 37. coco wapaniriridwa panopo coco sakuphula kanthu kuli frozy luk frozy drink ku m’chinji ndi k150 pomwe exotic k200 per half of litre 500ml,yes drink k400 per 500ml,super shake k450 per 500ml,mangos k150 per 300ml.MELINDA K250 PER 350ML.so luk pomwe COCO AKT K250 PER 300ML kkkkkk acoco ali m’madzi

 38. FROZY drink.it is a cheaper and gud flevour mmmm frozy drink is aproftable busness and my friend bought a car bcoz of that busness.KUCHIPATA NI MBWEEE KASI IWE WABWELA NIZAKUSHIMIKIRA

 39. Our fanta or bottle of cocacola is 300mls atK 250 to K500 depending on where you are buying yet frozy is 350mls averaging at K200 In this hard economic times people will automatically go for it Its high time soft drinks companies in Nyasaland think twice by making cheap and affordable brands otherwise one day one will not get suprised to see the local softies in Oblivion or extinction! “Welcome Frozy timwe zimenezi”

  1. Palibe kubwelera mbuyo ndi frozy guys chili chipani bwezi ntakachivotera! Team frozy! Nkhwiko yanga konzeka’KUKHOSI SAKANDIRA NCHITENGO koma frozy’ife ndi abwezi a frozy basiiiii

  1. Mutuwako chisilu mbuxi nyani galu fiti paja u only drink frozy pamoyo wako Griffin Wa Makaveli,amako alindi kireti yoti akamagula amatenga empty lokasinthisira

  2. Mutuwako chisilu mbuxi nyani galu fiti paja u only drink frozy pamoyo wako Griffin Wa Makaveli,amako alindi kireti yoti akamagula amatenga empty lokasinthisira

 40. Zokumwa Zimenezi Zikudyani Matumbo.Ndiye Wamwa Kale Ingopempha Chauta Kuti A Satanic Amenewa Kuti Asalowe Mu Mtima Mwako.

 41. M’bale Amakonda Kumwa Koma Pano Adasiiratu Chifukwa Adamupezesa Mavuto Monga Awa: A Malota Zoopsa Komanso Wabwera Zilonda Za Mimba.

 42. vuto ndi umphawi tilinawo mdziko muno,chifukwa izi zimayenera kupangidwa ndi ma company akomkuno like #sobo cocacola etc koma amangokakamila zodulazo,for example ku maiko ena ngt ku jon even cocacola yemweyu ali ndi magulu awiri otchipa(fongkong)ndi odula (original) munthu umachita kusiyanitsa malinga ndi mthumba mwako sabwezaso botolo

 43. The fact is in other countries they have low tax and production is high hence they start to export. Zikachuluka zimatchipa nde it’s easy to smuggle

 44. Za Satanic Zimenezi Maiko Ena Ozungulira Ife Adazikana Zimenezi. Mudzione Ngati Zili Ndi Real Country Code #. Mumwa Nawo Magazi A Anthu A Ku Satanic. Anzanu Ena Akunong’oneza Bondo.

  1. Not all itemz from abroad are smuggles, and are cheap not because they don’t pay tax koma generally ku Malawi kuno zinthu zimadula

  2. Not all itemz from abroad are being smuggled, & are cheap not because they don’t pay tax koma kunena zoona ku Malawi kuno zinthu ndizodula

Comments are closed.