Mutharika responds to Chakwera’s calls for his resignation

Advertisement
Lazarus Chakwera.

The Malawi leader Peter Mutharika has dressed down his political rival Lazarus Chakwera who is the leader of opposition Malawi Congress Party (MCP) for igniting calls for his resignation following social economic woes that have hit the country.

Chakwera is reported to have told his party members who had gathered for a political rally in Dedza last weekend that due to challenges that have rocked the country, Mutharika deserved to face the exit doors of presidential palaces.

Lazarus Chakwera.
Chakwera: Slammed by Mutharika.

He pointed out that the persistent power blackouts and water shortages in the major cities are a clear sign that Mutharika has failed to be a good leader for the country.

Reacting to the sentiments during a press briefing on Friday, Mutharika said he is to be in his office until the end of his term.

“And somebody said that I should leave the government, I want to ask him to take care of his political party first while his party is crushing,” said Mutharika.

On the electricity challenges rocking the country, Mutharika was quick to blame previous governments for not planning on the grid of electricity use in the country saying they never had plans to have plants that can generate enough power for the rapidly growing population.

Advertisement

131 Comments

 1. kma iwe busa opepera ngati iwe sinamuwoñe moti umuźe zoti áyendese bwino dziko bansi nkhani iziķhala imeneyo iwe ukazadwala mutu suzachira dikiĺa

 2. Inu mukadwala tchito imathera pompo anyani inu,wayamba kudwala ndiye,kodi muthu osadwala mungamuloze padZiko pano,mukagwele uko ndi chakwera wanuyo

 3. first ,chakwera must solve the problems in the stupid mcp then point afingure to APM. how can chakwera run agovernment yet he is failing to solve the problems in his own party? very shame

 4. Enanu ndinu zitsiru peter mutharika atengeso 2019 mufune musafune. kod chakwera yo analimbusa anasiyiraj ameyu ndiotembeledwa akadzalowa upresitent tizavutika so ilove peter muthalika my No 0994238773

 5. The difference between great thinkers and narrow thinkers Chakwera criticised policies Mutharika criticised Chakwera. Who is a great thinker here and who is a narrow thinker?

  1. Then you dont know what you are saying, who told you that being reverands, priests or bishops then you not practice politics? It seems you dont know what you are saying because all creation belongs to God even politics. Wodzudzula mapolicy ndi wodzudzula munthu as an individual wopusa ndi ndani? If ignorantly you dont know what you are ssying, please! Avoid commenting on my wall because i dont go for individuals, i go for policies said by individuals so idont need and miss your comments Mr. T. C. Gama.

 6. Dnt u think its time u vote 4 a malawian citizens?its time u stop voting 4 Foreighners,Peter is not malawian can’t u c dat,wake up guys

 7. zisilu inu ngati muli ma dolo osatenga dzikolo mulisogolele inu bwanji kwanu ku mpoto ndikuntchile kovesa chisoni even ma MP ochoka kwanu Ndi agalu okhaokha angonya. chocolate chawo ku area 9 uko. stupid mesa

 8. AAaaaaaaaaaaaa takuvani koma mau anga kwainu pali anthu ochuluka zed amene amapangitsa kut muthu awine kumwera pali maboma 6oti alipo otenga boma “//chiradz

 9. CHILUNGAMO:Ngati Achakwerawo adalephera kusamalira nkhosa za Yehova zomwe ndi zowerengeka m’malawi muno kulibwanji, ndiye ndikuwona ngati ndi zosatheka kuweta nkhosa ndi mbuzi pomwe nkhosa zokha zikuwakanika-ndinu mwana wolowelera,mwaononga chuma chambiri chomwe Mulungu adakupasani kuti mudyesere anthu ake koma inu mwatenga chumacho ndi kukapatsa ziwanda:RESULT-ndi moto

 10. Vote N Give Chakwera More Votes For Beeter Malawi N For The Better Future Of Our Kids Truly Malawi Is Sinking Dpp Can Be A Gud Party Koma Atsogoleri Ake Alibe Maso Mphenya Ndi Chidwi Chotukura Malaw Monga Momwe Bingu Analili Lets Vote Them Out Kut Asatitenge For Granted

 11. Mr Chakwera just waite 2019 elections, Peter will resign that time….if majority wish kikikikiki….but I don’t think if that thing will happen in 2019, but if Peter will step down in 2019 then Atupele Muluzi will take over, so Mr Chakwera U have more time to waite, 2019 will also be the leader of opposition, U will never stop opposing the goverment since u will never be in the goverment. George Chaponda is also waiting for that sit with petience, so Mr Chakwera stop dreaming for that sit!

 12. African politicians r greedy he can’t resign & don’t think that 1 day Malawi will be 1 of the best country when it comes to development never,just imagin our nation is in big economic crisis but our President is telling us that he wasn’t sick but he wasted a lot of our in America

 13. Malawi,we have to know hw the world going,what malawi is facing its globally now let us bring the solutions to change the challenges we are in,I would prefer to shift from Democratic governance to mornac. This has brought big changes in Asians countries,let us allow peter to rule forever

 14. Tisamanyoze atsogoleri koma tizisekelera zopusa zomwe? Ngati sakuchita.bwino tikuenela kuyankhula infact ndi chitsilu ndithu bwampiniyu.anthu ena kuzolowela kusekelera zopusa mxiew!!

 15. Ndale a Malawi sitizidziwa timangofuna kutchuka basi.Peter walakwa ciani?Bible limanena kuti tizimvera atsogoleri athu osati kumanyoza monga timacitiramu.GOD will not heal our country ngati tipitiriza khalidwe lotero

 16. The main challenge we have is we vote for only old people if a person is 70yrs above is in extra time within 2yrs gone.

 17. Chakwera ziwa ichi, upite kwa John Tembo ukafunse kuti. Impechmemnt inayenda bwanji ku paliament ndi Bingu, 2005 pamene ali ndi aphungu 6? Ndikhulupirira kuti, akakuyankha bwino lomwe kuti samala Bingu anamutumizanso nkulu wina ku sukulu chifukwa cha nkhani ngati yako yomwe. Akakuuza kuti samala, usapitilizenso kulankhula nkhani imeneyi chifukwa certificate yako ndiya ubusa.

 18. inu tikuti nkuluyu ndiwodwala tamvetsetsani musamuvere matendawa amugwiraso ubongo ofunika abwerere kuchipatala akamuwuike bwinolomwe vuto ndamene akudwazika matendawo sangamawawuze matenda kuti adzilimbitse pamene muthuyo salibwino pakufunika madotolo owonaso zawubogo ngati antaba amuwunike bwanphiniyu

 19. Kodi munthu ukamadwala, bwanji osangovomereza kuti ine ndikudwaladi, ndisiyire wina wake mpando uwu, ayendetse dzikoli? Sikuti ndi za ufumu wapa mudzi izi.

 20. Neneli onyenga uyu, galatiya, busa wanji othamangitsa khosa? H z failing 2 ru hs party wth patriotzm nde angalamulire dziko lonse.

 21. Changobwera kumene kuchokera ku chipatala mutunso suukugwira, kusiya ku solva mabvuto a mdziko kukalimbana ndi Chakwera. Utsilu eti? Manyi ake

 22. Pena pake mutharika amalakhura ngati mwana wakuprimary. Zomvetsa chisoni ndi anthu ena omwe amamuombera manja. Iye akulimbana ndi chakwera president wachipani. Baba tasiyani usilu mukupangawo tayambani kukonza zinthu dziko muno, mavuto ali phwiii. Chilowereni boma chanzeru mwapanga ndikupita kwamerica kukadwarako ndikuononga misokho yaife.

 23. Ochakwera paja achigawo chapakti amalankhula choncho.Kulimbikila zaziiii akuwuza kuti sangathe kulamula.Mantha alithoooo kuopa 2019 kuti zingavute maka munthu ameneyi.ndichipani ichi cha DPP sindizadutsa.Mumafuna Chilima wanuyo kuti muzamugwetse mamawa mwalephera.Muntharika mufune musafune akuzakuwumbuzani kolapisa 2019 mpaka 2024 pozafuna kusiya azamenyala nkhondo azafuna kutenga mpandoyo mpaka 2028 mnyaaa simunati.DPP ndichipani chokhacho chingalamule Malawi enanu muzitsutsatu basi

  1. Guys Tizipanga Makani Moganiza Poona Momwe Zilili Zinthu Pa Ground Its Not We Hate Dpp Or Muthalika Koma Ulamuliro Wake Tangonani Momwo Moyo Ulili Like In Hospitals, Admark No Maize, Education N Fees Hikes, Blackouts N Water Shortage Worse Than Before, Zinazo Ndikumbutseni Nokha Taonani Kut Malawi Akupita Ana Athu Azapeza Malawi Otani? Sizitukwana Apa Lets Build Malawi Together As Malawians

  2. ine ndikudabwa chimene mukunyozela Peter,,kodi iyeyu ndi mulungu kapena munamuona kuti amagwetsa mvula? kukakhala njala ndiye kuti mvula siyinagwe bwino,,ngakhale nthawi kamuzu ife tadyapo chimanga chofira chimene ku America amadyesera Ng’ombe,,kambani zina.

  3. Nanga Mankhwala Mzipatala Ikufunikanso Mvula? Maphunziro? Katangaleyu (cashgate) Kusowa Kwa Ntchito Kusayenda Bwino Kwa Malonda A Fodya M’misika?

  4. Kkkkkki wina akuti ndne oxazindikila chifukwa cha APM.kdi inu amene mukut mfweeemfweee watani peter zinthu sizisintha nthawi imodzi dikilan muone kusintha pompano

 24. A chakwera mwasowa chokamba et akatula pansi udindowo ndie kut zinthu zisintha?kupepera chakwera pezani njira zothesera mavutowo kutula pansi udindo si solution yothesera mavuto koma kukhala ndikukambirana komanso patavuta bwanji sitingakuvotere satana iwe kuthawa ubusa kupita ku ndale mulungu wakwiya nawe kwambiri uzakhala opposition mpaka kale plus apo ukulephera kuthesa mavuto amuchipani chako ndie ungakwanise dziko iwe

 25. I doubt if he was thinking when he was altering these words. He cant compare problems rocking mcp to the problems malawi as a country is rocked in. Chakwera is just a president of the party while him is a state president. Pena mukuluyu amayankhula ngati mwana and its just petty that omusatila amaona ngati wayankhula zanzeru nkumaombera mmanja, he cant even think that even those in mcp calls him their state president. Mulungu azayankha tsiku lina tizakhala ndi mtsogoleri osati izi zongopachikapoyi.

 26. Av Nothing With Leadership But Problems Malawians Are Facing,amene Sakudziwa Mavuto Ali Kumalawi Ayamike Wammwambayo And Anthu Anadakukhosi Nkhani Yautsogololeri Wabwino.Umboni Ndimomwe Ovota Akuchepela Masiku Ano.

 27. Kodi bwanji achakwelawa angolimbikila kuti apresident athu okondedwawa atulepansi udindo bwanji osadekha mpaka 2019 akuopa chani? Kodi mavuto amunthu owathesa ndi president? Ayi mulungu ndi amene amathetsa zowawa.ngati iwowa anatula pansi ubusa kodi ndiye angathe kuyendetsa dziko?mmmmm ayi anaonetsa kusakhwima mzeru muli ngati yona mulungu ana nyasidwa nanu Achakwela mufunse atembo akuuzani shameeeeeeee!!!

  1. mcp ikut chakwera atule pans iye akukana ndie akufuna peter atule ? amangodzipopa popeza kuononga ndikophweka ngat kuendesa boma angakuthe

  2. what people are asking for is provision of services and chakwera at the moment is not in that postion but Apm. so Apm is the one failing us.

  3. yohane you want APM to be giving you money every month so that you will say he is doing good? Or wat?
   what you should know is that, not the president can change things ln our every day life,but God in haven can.
   pray to God he is the one bringing a change in mans life

 28. Munyumba mukakhala bambo ndi mai ngati wina akuyala kuti nthawi yakwana tigone ndipo wina akuyalula kuti tisagone ndinthu munyumbamo simungapezekemo mwana.

  1. akulu akulu lets be serious.. u must differencitate intwlligence am leadership skill.. peter alibe leaderahip koma intelligence nde amalaiwi kutengeka coz he is rich munavotera..lets not blame the leaders koma we ourselves are ignorant.

Comments are closed.