Malawian conjoined twins die at KCH due to blood shortage

Advertisement
conjoined-twins

Conjoined twins that were born over a week ago at Nkhotakota District Hospital have died in the course of a surgery to separate them, Malawi24 can report.

conjoined-twins
Dead!.

The twins died few hours before surgery to separate them at the Kamuzu Central Hospital (KCH) in Lilongwe.

Spokesperson for KCH, Mable Chinkhata confirmed the death.

According to Chinkhata,kids were supposed to undergo surgery on Wednesday but the process was delayed due to shortage of blood suiting their blood group.

“The twin needed about 200ml of all negative blood group but due to the fact that the hospital did not them,we failed to carry on the surgery”,querried the PRO.

It is reported that the twins died as they were struggling to breathe and efforts to resuscitate them failed.

Advertisement

221 Comments

  1. Tikukhala Dziko La Tsoka,atsogoleri A Tsoka,umoyo Wa Tsoka,chakudya Cha tsoka Ndiye Ife Titani? Tingoti Amene Adalenga Anawa Alandireni Ambuye Poti Sadziwa Kanthu Ndipo Muwalandire Monga Mwakufuna Kwanu Amen!!

  2. Zimenezo Ndiye Zopusazo. Munthu Amapangidwa Operation Mukudziwa Kuti Pali Magazi Ochepa? Ngati Sakadatha Akadapempha A Mabungwe Apite Naye Kunja Osati Manyaka Akunowa Ayi.Poti Mavutowa Akuyambira Kumtunda Mpaka Kothera Kwa Dziko La Malawi Ife Tilibe Chonena Chifukwa Umoyo Anawo Akadakhala Ndi Atsogoleri A Maiko Ena Sibwenzi Tikumva Zopusazi Ayi. Ndiye Zatero Ayi Tikukhala Dziko La Tsoka,chakudya,utsogoleri,umoyo,kuyenda Tikukhalanso Mwa Tsoka. Zaoneselatu 371 Ikugwira Ntchito.

  3. Zimenezo Ndiye Zopusazo. Munthu Amapangidwa Operation Mukudziwa Kuti Pali Magazi Ochepa? Ngati Sakadatha Akadapempha A Mabungwe Apite Naye Kunja Osati Manyaka Akunowa Ayi.Poti Mavutowa Akuyambira Kumtunda Mpaka Kothera Kwa Dziko La Malawi Ife Tilibe Chonena Chifukwa Umoyo Anawo Akadakhala Ndi Atsogoleri A Maiko Ena Sibwenzi Tikumva Zopusazi Ayi. Ndiye Zatero Ayi Tikukhala Dziko La Tsoka,chakudya,utsogoleri,umoyo,kuyenda Tikukhalanso Mwa Tsoka. Zaoneselatu 371 Ikugwira Ntchito.

  4. The procedure was not successful. Not some stupid comments.. U don’t even knw a damn about surgery and ur busy insulting doctors.. The government..

  5. Abale Mwa Ambuye,tiyen Tiphunzire Kuvomereza Zinthu Zikachika,rmemba De Bible Syd,pachilichonse Yamikani Ambuye,end yense amene anabadwa akuyembekezeranso kumwalira,imfa siimathawika abale coz nthawi yamulungu ikakwana palibe angaibweze.Mulungu Akukhululukireni Nonse Amene Mwayankhula Udyo Kamba Kopsa Mtima.Tisaweluzane Coz Kuweruza Ndikwa Mulungu.Mizimu Ya Anawa Iuse Mumtendere.Amen!

  6. Very sad koma god knows akanakhala kuti anali ana amunthu oziwika pano mutaitanisa ndege kupita ku maiko aluya koma poti ndi osaziwika mwapanga zofuna zanu ok nthawi ikubwela

  7. Ooo pepani, kunonso Ku SA Boma ndi akubanja Ali pamadiscution kuti apange bwanji coz vuto ndilomwero chaku western cape uko kwabadwa Ana olumikizana pachidale koma vuto ndiloti kuti aalekanise m’modzi ayenera kumwalira chifukwa akugwilitsa ncito chiwindi chimodzi ndiye madotolo akudikila yanko kuchoka kuboma ndi akubanja kwa Ana, kuti atani.

  8. Why not gov helped to send them to other countries for good service through the minister of healthy???? It means muntu akakhala osauka mulibe nayo ncito eti? I’m sorry may God Wellcome their souls in heaven.

  9. Anawo anali ndi magazi ochepa kale ndipo analinso asanayambe kuwathandiza anthu mumachulusa zokamba mukadwala madotolo ake amakuthandizani ndi omwewa nde mukuwanyozeranji

  10. the twins have died due to the inavailability of blood(group O rhesus negative which is scarce) before surgery NOT during the operation! it seems anthu ambri mukungo commenter osawelenga nkhaniyi bwinobwino…

  11. Amayi pepani ámálawi enafe tinabwadwa oģwirá ntchito anaĺi omwewa mpaka pano tiĺi nďimoyo añakamwalira ķu uķ simukanatokota chonchi shame palibe munthu amapanga moyo only god emweyo atothoze banja loferedwa i proud to be malawian

  12. Mesa chamma 10am lero amat analephera kuwapanga oparation dzulo ndiye amat akamaliza ku KCN lero masana, so which iz which??? Penapake2 mukutionjeza aNews24

  13. R I p. Ambuye Khalani Ndi Banja Lokhudzidwalo, Ngati Ali Satana,kuweluza Ndi Kwainu.Afungatileni Ana Anu,Zonse Tizisiya Mmanja Mwanu AMEN.

  14. Eish,,we don’t have enough equipment in malawi for serious operation,on top of that the doctors are not often dealing with kind of operation that need well trained doctors

    1. its nt the doctors’ fault. the operation did not take place sir & this was because of blood (group O rhesus ,negative which is scarce)..the babies died of cardiac failure due to severe anaemia (don’t trust this site

  15. NDIFE ALENDO PADZIKO LAPANSI PANO : ANAWA KWAO KWATHA, MOTO UMAYAKA KOMWE KWASALA TCHILE. NO JESUS NO LIFE. >>>>> 2016

  16. Tipaone bwino bwino pamenepa amafuna ayesele kwa anthu timayesela kwa zinyama. Izi zimayenela kunja izi akanakhala mwana wa munthu wa m,boma bwezi ataba za misonkho yathu kupita kunja koma popeza ndi osauka mwapha osalakwa musamale

    1. nt the doctors fault cause anawo amwalira cfukwa cha severe anaemia before the operation…and the blood that was required is O- which is scarce…so maybe MBTS fault

  17. Bwanji osatumiza kunja? Inayamba itakhalapo successful operation yoteleyi kumalawi? Mmafuna muyeselepo chifukwa ndi wosauka.koma the gvt spends millions on nkhalamba zofa kale

    1. I don’t understand wen u say “nobody ever deserve to die” bra, death is there, wheather we like it or not, the pair u ar talking about was just lucky, just like here in Malawi, there’s also another pair somewhere that survived the same operation, wat if the operation of that pair u ar talking about was a failure, do u think pipo of that country would stand on top of the mountain and accuse the doctors of incompetency?, its a complicated operation we ar talking about here, its life or death

    2. these twinz deserved to die than leave a miserable life, Im against this part coz once you are born,you deserve to live regardless of your physical ability.Its only in our country where everything is awkward.I dont mean we wont die but circumstances sorrounding your death is what we are talking about here.Sorry my grammar is not ok…english is not my language.

    3. Nyapapi iwe bakha tokhwetokhwe kaligondwe gokhwiro iwe wandikiya kwambiri,,They deserve to die.what if those innocent children you were the father and someone saying those how would you feel ? instead of feeling sorry for those innocent soul because of poor management in the hospitals of Malawi and what you to know is that when the doctors want to take a serious operation that they always make sure that every thing is set ,not as what they are saying blood shortage…Poor malawian we will always be killed as cockcroaches ,,these greedy politicias are out there enjoying with their families our on money not donating for this operation to done by experts who know their work not these trainees…Am really ANGRY with you for your heartless words *#-+ Mtumbo wako matongo ako uli ndi ana koma iwe ?mwina umadya maliro eti?? Gojo iwe umakudziwa kubala ?? Mutu ndi machende ongodzadza ndi MAMINAwo moreover Machende amako galu iwe kuzolowera kumwa magazi eti nde upite ukatenge matupi a anawo ungochita ka Braai ukhwasule munthu opanda chisoni Phwala lako mboli yako Olivian Oliva Twist Pagone …

  18. Stupidity is writing your comment based on recent comments or based on a story of some headless chicken of a journalist, who said the kids died cuz of an operation cuz they were not operated… I repeat, the operation did not take place.

  19. asatinamize its organized deal in a case dat they share never ever separated organ why doin surgery in absence of blood

    1. the kids were not operated,coz they were still waiting for mire blood to supply the kids before the operation & the kids were aready anemic.Im sure it was God time to make them die.

  20. Maybe its Gods plan,this is the first case in our country.if God says tdy is ur tym to die ,no matter hw many qualified doctors are infront of u,but u wil surely die bcoz its ur tym

  21. zowawa kwambili. oroso kunu ku SA ziliko ana anabadwa mwezi wathawu koma ophatikizana chest nde akuti ngati kuli kotheka makolo avomele kuwapatula koma yimozi mwa anawo amwalila after operation nde akudikila makolo kuti ngat amvomeleza kutero ma doctor apanga mwatchito yao. but zimakhala zowawa kwaife monga munthu wamayi kusunga mimba mpaka miyezi 9 koma kungovutika pachabe so sad. Rip

  22. Zandikhudza kwambiri ndikaganizira mayi nzanga kungotsala ndi bala la operation lopanda nalo malipiro umalimba mtima ukamaona chiphyera nkumamuonanso mwanayo…zandikhudzaa kwambiri ana aja sanaenera kuwapangira operation kuno…anaenera anakanwatumiza kumaiko anzanthu amene amakwanitsa ntchito imeneyi….Autse Mumtendere…komanso tiyeni timupemphere nzathuyu amene waluza anawa…amene muli naye kufupi mpatsen mau a CHILIMBIKITSO…

  23. Akadakhala kt adali ana amunthu wandale wotchuka kalekale sizidakafika potelepa. Amalawi timalimbana kufunira zabwino anthu omwe alindikuthekera kale oti zoterezi zidakawagwera adakatha kupita kunja ndi ndalama zaboma kusiya zawo zili phwiiii… Malawi nyasii kwambiri!!!

  24. Ine ndikamva kuti awawa ndi a Dr kapena Professor so-and-so, sindimanjenjemera. Ena ndi awa adakwanitsa kungotchola nthiti ya Daniel Phiri wa. Ena ndamene akulephera kuyendetsa dziko wa.

  25. Wat i know munthu sapangidwa operation palibe magazi okwanira how come that the doctors operates the babies while there was insufficient blood? its lie you have killed ana thanzi ngati amenewo. God will punish.

    1. Akubitsa anawapanga Operation koma chifukwa choti awapha. Ana athanzi akamwalire lero? Samamwalira dzulo bwanji? Mukaphunzilire pawanawa zoona inu anyamata aku COM

    2. God will not punish anyone here coz if they made a decision of operating them, it was for there own gud coz the survival rate of conjoined twins is slim becuz of their physiology. So stop blaming doctors and do urself some research

  26. Ndiye zachamba zimenezo osangoti mwalephela kuchita opaleshoni bwanji,madokotala akumalawi osaziwa ntchito yawo koma kukadakhala kupeleka asipline ndi panado basi,kulatila adwala.

  27. Eeeeeee u Doctors is this true blood shortage?how many litres would these kids use in 4hours?may their soul rest in peace

  28. Musaname kuti anasowa magazi pakuti ukadaulo wavuta apa, mumapanga ntchito yoti mulibe nayo zipangizo bwanji?cilungamo ndichoti afa kamba kotaya magazi pochokela ku opaleshoni inapangidwayo, osati kusowa magazi, iyah muuza ana? Fotseki.

  29. Its so sad may their saul rest in peace, this was serious operation that it really not be done in malawi it was surpossed the goevernment to help to donate money so that it could b done out of malawi

  30. Zonse ndi a Escom, anazimitsa magesi, kodi company yopanda solution ngati iyi ikukhaliranji paka lero? igulisidwe sikutipindulira, ma bwana awo anakachosedwa ntchito coz samatha kupite ena, pano mukuti madzi achepa mvula ikagwa muzizati zinyalala zavuta, wake up Escom mxuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuuu

    1. Hahahahahaha????!!! Ndasekaaaa ngati zabwino tu koma ayi ndithu, moti pena ndimati Malawi ndi dziko lotembereredwa, ngati ndimalakwitsa, Yahovah andikhululukire, coz zimachitika kuno ndizomvetsa chisoni komanso zoseketsa… everything poor indeed. Pena kumaona ma citizens ena ngati amisala coz momwe akuonekera;osasamba komanso kusowa zovala zabwino. Malawi ndi dziko lomvetsa chisoni, literally, to an extent that you could cry. Koma poti amati Mulungu salakwitsa, we still give thanks for our land Malawi.

    2. poor doctors!? what role did they play in the death of the babies. the operation was not done, so do u blame the doctors for blood inavailabilty?

  31. This is lack of expertism I am sorry for the death of these babies and am sure suppose the were born from a family of prominent politician the government could use government money to take them to an expert outside Malawi. May their Souls RIP

  32. Shortage of materials in hospitals of our that’s leads to lost our familys and friends.government take note on that issue pliz Rip

  33. Sometyms zipatala zakwathuk zipangizo ndizochepa coz vuto ngati ili likadadziwika before anawa asanabadwe n akanapenza njira yoti anawa athe kukhala pake-pake, so sad.

  34. Due to blood shortage or because it was a complicated case?am sure they had to make blood available b4 surgery. Dont misreport these things

Comments are closed.