Bakili Muluzi’s corruption case adjourned again

Advertisement
Muluzi

The Blantyre high court has again on Wednesday, adjourned to next month the K1.7 billion corruption case involving the former Malawi president, Bakili Muluzi.

Muluzi is being accused of squandering public funds during his era amounting to K1.7 billion and his case has been in court over ten years now.

This time, the adjournment follows an application by Muluzi’s lawyer who asked the court to give his client enough time to study the evidence presented in the court by the Ant Corruption Bureau.

Bakili Muluzi
Bakili Muluzi : His case still stalls in court.

According to ACB’s legal representative, Clement Mwala, the state evidence which Muluzi’s lawyer, Tamanda Tchokhotho says they need to study it more, include bank statements and all other documents.

“We have filed and submitted to the defense to affidavit. One complying with banker’s evidence where an official bank is stating the source of the document from the bank where we are relying on.” Said Mwala.

However, Tchokhotho said the documents which they have been given as evidence of the government, will require more time to make a forward decision on the matter.

Recently some political parties in the country have expressed concern on the dragging case saying the delay to conclude the case is hugely costing the government.

Muluzi was first arrested in 2006 and again in 2009, on charges of stealing millions of dollars in donor funding, and many hailed his arrest as a bold move towards fighting graft in a country that’s been held back by corruption.

It has been alleged he diverted donor money from countries like China, Libya, Morocco and others into his personal account.

Advertisement

180 Comments

  1. Kodi amalawi kukonda kuwoneka azelu pobisa u chitsiru wanu bwanji one millon ndalama yochepangati imeneyo aaa alamula anthu angati kuchoka pa muluzi

  2. mukulimbana ndiamene sakukuyankhani komaso mukusaka popeza simunadye nawo enanu munatenga ndalama kukamangila univesity kwanu panthayi yajoice munadyera limodzi lero upretend to be honest kwa apm ana anjoka inu leave muluzi atsogoleri akwathu sadzapezeka wabwino

  3. tamusiyeni muludzi timaja ñawo zi ko lotse limaja bwiño ndibakili munene dzawa awa alomwewa, ķuzolowela kubitsa mbewa komatu kuvinidwa kwabwiño mutu umagwila bwiño ntchito akutibela galuyu

  4. Just drop the case for him why you still lukin on that? last tyme were hearing that he dont have a case to answer now you say the case is adjourney again which case are you tell pipo ? Bwanji osafufuza ndalama zambiri zija mkulephera kuitanisa Jb msiyeni mluzi anamenyera ofulu wa ziko

  5. njila zobela ndalama mwazipezano mukungowononga ndalama chikhalileni mukuziwa kut mulandu umenewu simunngaukwanise kkkkkkk dzuka malawi

  6. A real citizen to rule malawi Nanga ma president osankha kulankhula chichewa wa tiziti ndi nzika za dziko la malawi? Mwina dziko la malawi kugona mpaka alendo atatu kulamulira dziko nzika zeni zeni zilipo leave Bakili alone

  7. Am feeling bad with this corruption case of big man #muluzi” What is going on with our country malawi milandu ya ena mukumayipondereza pamene ya ena mukamavumbula eishhh!

  8. Kuba ndi kuba zilibe kanthu kuti waba pang’ono komanso k1.7 billion si ndalama zochepa kumusiya ameneyi ndi kupereka mpata kwa ena kuti azibabe kwambiri. Komanso onse akukhuzidwa ndi kubedwa kwa ndalama za m’boma kaya ndi cash get kaya ndi aBingu anabanso amangidwe basi chifukwa ndalamazi ndizathu a Malawi, nde sindikunyengera kuti ndi ndani amamva kukoma akamadya ndalama zathu anthuwa ife tikuvutika. A Malawi tisamapuse pena ndalamazi ndizathu timaziphwekesa chifukwa timati zabedwa ku boma, koma ndithu ndizathu ndalamazi. Anthu amatisekatu ife ngati sum’maziwa amati Malawi is a village, ine nde ndisaname zimandipweteka pokhala ndine m’Malawi. Pali munthu winawake ndiwaku Zimbabwe ndi yemwe amatelo nde osamasekelera zopusa, aaaa basi musiyeni kkkk koma, zili ngati kukubera nyumba mwako ka, inu mungamusiye wakuba mutamugwila ku nyumba kwanu atakuberani? Anjatidwe basi onsewo sindikusankha osewa ndi mbava zokhazokha, nde enawa atengere chisanzo pa iyeyo zikomo.

  9. Osalimbana ndi cash gate ya fresh kulimbana ndi Bakili Idiots in gvt shit,Leave Bakikili alone iwe Ptr or else,olimbana ndi Bakili adzisowa

  10. Akuyenera khuthana ndi onse omwe anaba ndalama zaboma starting from Peter and his late brother.These dudes stole a lot of money than the money they claim, by the way the government should find out who murdered Issa Njaunju first if they are on a right path.

  11. Onse a dpp mbuzi owasatiraso mbuzi ma court onse mbuzi za anthu peter ndi gulu lake mbuzi iweso zakubowa mbuzi ya munthu ngat mulip ambir mbuzi za anthu leave muluzi and conctrate on changing malawi so many prblm busy spendin mone for noting mbuzi

  12. musiyeni muluzi ntchito yakeanapanga imuchitile umboni plz musiyeni umbulibasi ndi jelasi ndiomwe wachuluka kwathu kumalawi zausilu. …zapatumbo notu mukupangazo zatitopetsa panyopamako amene akulimbanandi bakili kusavinidwa ndikomwe kukupangasa bakili tutsamasakha thundu kapena chilakhulo ayi amathandiza winaaliyese koma nyapala iwe wabwelawe ufamosa ziwikabwino usaganizenga athuakukuonandi diso lachikondi akukuonandi lausatana pomaliza tupele 2019 ali boma ndiposo osakaika …zausilu Patumbo pako

  13. Sitinyoza boma komano kukupitaku tizinyozano mukulimbana ndimunthu sanalakwe osayimba milandukaye AKUMABA AJA BWANJI MUSIYENI MULUZIYO MENE AMALAMULILA MUJA ZIKOLATHU LINO LIMAYENDA BWINO KWAMBILI EVEN NDALAMA INALI YAPHAVU KULOWA WALOWA BINGU ZITHU ZINASOKONEKELA pls MUSIYENI MULUZIYO

  14. Ngati panali president wachifundo okumva zidandaulo za amalawi, ndie DR. MULUZI. Inu ndie mukulimbana ndimunthu oti anapangisa malawi kukoma? Nanga izi ndie chani ndalama zili biiiii ngati koma akuti zikugwila ntchito……lorani kuti mwazi wanga ukhale petrol yoyendelasela dziko, koma mutsiye muluzi…#cashmoney

  15. UMBURI Wa athu ophuzila. Kuti mufike pamenepo ndi ndani ? Osayamika bwanji kuti munalowa boma chifukwa cha muludzi.bwezi titalowa ife MCP. Ndakwiya nanu . musiyeni muludzi. Pano murine magetsi osaisova bwanji mburi za ziko shame to you

  16. multipart is war.luk at Britain there isn’t issues lyk multipart or even elections, let’s luk at USA they hav a system of gvnmnt where 2 candidates compete 4 de sit of president , but Luk at most African countries we multipart system we also share common problems (multipart)

  17. nkhati zakuvutani sakilani zina zochita not kulimba nzopanda pake,mbala zinaba dziko lonse mkudziwa ndiye koma osachitapo kanthu ndiye mukalimbane ndizomwe sitinazione? ndinu agalu mbuzi zawanthu mulekeni muluzi ausumane poti nthawi yake tinasangalala not nthawi yafinye achabechanu.

  18. Mukumputatu mdala Nelson makolija mapeto ake mutha ngati makatani.mukuwasiya dala ABITI MALOKO NDI CASHGATE YAO.2 NDUNA ZAPETER, anga ndimaso kuyang’ana inu

  19. Ngati mukukanika mumuzenga mulandu munthuyu bwanji 0sang0musiya????? Milandu ya anthu enawa yayenda msanga bwanji???? Examples are: kasambala, man0nd0, kumwembe, lutep0 and s0 many bt Muluzi mukutiw0n0ngera naye nthawi and g0vernment res0urces.

  20. Kodi inu aboma chomwe mukupindulapo ndichiyani? Potimukupitilizabe kuwononga ndalama zaboma bwanji osangomusiya kumuyimba mulandu muthu ameneyu fuck zanuuuu mwamva

  21. wat z 1.7bilion? mulibe ulesi ndipo simumagwa m’mphwai. kod Atcheyawa mukuwapezerela chifukwa ali mmalawmuno?

  22. Zaziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii lero limenelo ngati zakuvutani tangokharani pansi malo movomereza zomwe muonengela pomayenda kunjako mkalimbane nda achalume ku phsimbiliza etiiii,,,,,

  23. Tangozitayani nanu monsemuja mukhululukileleni big man wathu iye samadya yekha amathandiza ovutika koma inu mwaba zambiri mpaka pano mungodya nokha anthu opanda chisoni inu Bakili amapeleka kwa aliyense koma inu kungoti Kakaka musiyeni muthu asafe ndi ntima mwanva!

  24. Mulimbana ndi amuluzi aaa,mmalo mokoza vuto lamagetsi isah,cholinga mummange,dzakukanikanitu apa bwanji mumangeso mtembo uja wa 63 billion, fuck up

  25. Zapamtumbo zanuzo ine ayi ……kod mumafuna kut munthu azingokhara osawuka??bwanji osakhoza vuto lomwe liri mm’dziko muno mxm

  26. Izitu akupanga dala, pamapeto pa zonse Mlandu udzapezeka kuti ulibe maumboni, zikatelo boma lidzamulipile ma Million Bakili, koma mbamva inu?? Mxiewww!

  27. We all know how it works. Don’t we?? In the end its gonna be like “there was no evidence” so why wasting tax payer’s money? That’s democracy for us. Azungu pretty well knew what they were actually forcing down on our throats. They know very well only a strong hand can keep a black man straight and sober. A straight and sober nation means a progress in development. Azungu had to weaken our government systems to make us drunk in the name of democracy to a zero progress. Any president with his ministers and freinds will always loot during their reign in the name of democracy. Democracy was a dose prescribed to Africa to keep Africa asleep!!

  28. M’mene nkhaniyi inayambira muja osangoyithetsa bwanji? Musatiputsitsepo apa nkhaniyi inatha kalekale. Bakili sangamidwe Atupele ali m’boma.

    1. 1.7 billion compared to 577,21 and I dont know how many billions now!who fucked up the most?who is fucking who?DPP woyee!2019 mbobillions!

    2. ur ryt bro @ lameck……surtee……ngati uli wakale litsate ziko kuchokela pamene analisiyila kamuzu kufiki pamene analisi…ila bakili kunali minda ikulu ikulu ku mulanje (fame)yomwe kumatuluka mntochi malalanje chimanga tea fodya and etc school inaliyolipila koma maphuzilo anali ndiphamvu zipatala zolipila koma makhwala samasowa…..(zomwe zimathandiza financial mdziko)..atatenga boma muluz anathetsa zonsez kumati ndine mnyamata wapatoun sindilongodola zolima ok kwacha ndi landi nthawi yakamuzu ndi sa rand ina k1 ipanga r2 bakili anaichotsa konseku nkuisiya pa r1 to k21 bingu anaibweza kufika pa r1 to k18 munati ndiopa mpaka kumupha…….matafale .achikauma . a stambuli alikut ndi ena ambili kuvetsetsa kovuta koma palichilungamo tien tivomereze

  29. mungolemeletsa ma judge ndi onse ogwila ku court basi.mbuzi za anthu inu.musiyeni Muluzi adye tomwe anasolola.inunso womolani muzizadya mukaluza zisankho 2019.

  30. Umenewu ndiye ndi ugalu tikukanawu,, osawamanga acashgate omwe mukuwasungawa bwanji? Ndiye mukafukule mtembo wa bingu muumangeso. Poti naye anaba iya, msiyeni muluzi apume he deserve respect

  31. Koma ngati dziko litha nsanga liyamba dziko lakumalawi kutha kkkk kwachuluka mbuli .mukulimbana ndi muluzi koma mukapita mmanyumba mwanu mugona ndi njera, musowa madzi, magetsi anakuzimilani karekare .tamusiyani muluzi plz

  32. Sickness to justice minister. Money ur spending on this case is almost more than wht he steal. Why we are so brutal to this attitudes? Can u send muluzi free ? Let him use the money to develop others since he is a gver. Ur blocking him from gving ,pls

  33. Kikiki poor Malawi. I just feel shame to be Malawian sometimes. What kind of politics is that? Just want to humilate and strip good respected pple. When we talk about developing our country its Zero. But our country is famous of arresting any politician who dont agree with current administration. Nthawi yaBakili tinkadya kukhuta. Malonda mbwembwembwe. Misewu milato inali kuoneka. Ntchito zake kumachitira umboni. Koma lero they cant point 1 project. Does this going to bring electricity,food,infrastucture? Kaya

  34. acheya akhalebe moyo.presdent osayang’ana nkhope.nsanje mpaka kalonga.anakaponda pa kande mumzinda wa nkhata bay 2 times.palibenso prensdent adzafikila pa acheya.ine waku nkhata bay ndikuti acheya akhalebe moyo.inu mukungotha nthawi yanu.billion ndi chaniso apa.ya galimoto imodzi potche.

  35. Its jst the waste ot tax payers money.hw many years ar they going to finish this nosense.birds of same feathers flock together.

  36. With his son even confusing govt on land matters and the govt goes by this, do you expect the case to end? Govt will definitely pay him handsomely at the end of it all

  37. NKHANIYO AKUIKAKAMILA KOMASO IKUSOWA MA UMBONI. KOMA ADPP ANABA NDALAMA MPAKA DZIKO LATHU SANZA ZOKHA ZOKHA NDALAMA ZINA KUMAMANGILA MANDA KOMA ABALE MALAWI AMOTO NDITHU.

  38. 63billion,,,Bingu.JOYCE mabillion…..ndikumalimbana ndi 1.7 billion kodi 63ija anadya ndindan wat l knw palibe amapita ndi ndalama kumanda jb z also alive bt mwangokhara chete government kuphwekera khalamba yomwe inathandiza kumenyera ufulu pamene enawo mukungozisiya aaahh gvnmt deal izikhara fair muluzi mwamulanda zithu zingati enawo maziko aja anamangira chani??

    1. Kusiyana kwa nkhani iyi ndikoti 1.7Billion ikukambidwayi, Bakili anathyolera nthumba mwake. Pamene JB mukulimbana nayeyo ndalama inaonongedwa mu ulamuliro wake. Muzitha kusiyanitsa

    2. Man ngat chizungu chimavuta zinazi muzingozisiya look bho bho anena kut involving bakili muluzi anena kut taken by muluzi ngat osamafuna kuchenjera mwamva come again ndi boma lakoro..

  39. mulandu mpaka zaka 7 koma sukutha ndiye ukazathamo azakaseva ukaidi wa zaka zingat pot zambiri zadusa kale koma president wa lomweyu sazathekaso mpakana iweso peter umwalira uwusiya mulandu umenewu ndat mmene anachitira bingu akulu ako aja

Comments are closed.