Police arrest activist Billy Mayaya

Billy Mayaya
Billy Mayaya
Mayaya: Arrested!

Malawi Police officers in the capital Lilongwe have arrested human rights activist Billy Mayaya for taking to the streets this morning in protest of persistent blackouts and water shortages that have hit  the major cities of Malawi, Malawi24 can confirm.

Mayaya disclosed that the anti-persistent blackouts and water shortages demonstrations were set for Tuesday despite Lilongwe city council and Malawi Police advising him to reverse the plan during the meeting held on Monday.

He asked demonstrators to bring candles and charcoal while they are in black cloths.

However, the police on Tuesday called off the demonstration by arresting the the organizer Mayaya arguing that he defied the police and city council.

The police are yet disclose the charges levelled against him.

Mayaya was set to start from Area 18 roundabout to present a petition to the authorities over the blackouts and water shortages.

Advertisement

315 Comments

 1. Marching coz magetsi akuthima kufuna kuchuka chani population is too high mapeto ake kudula mitengo basi osalangiza anthuwo bwanji kuti atsiye kuberekana ndikanakhala wa zachipatala bwenzi mkupanga compulsory kulera basi eee zanyanya munthu sali pa banja koma mwana sali pa ntchito mwana why Malawi akathima ndiye wina sakuyendesa bwino dziko kuiwala kuti tachulukana mmmh

 2. Kwina kuli konse kumakhala malamulo whether you CSO leader mkulu uyu anaudzidwa ndi apolice kuti atsinthe siku la mademo koma anakana or ndili ine kumulowesa mu chitokosi basi ukamacha ndiye ayaka akathima umayasa generator ndiye ukukatenga oyasa kandle kuti tiyeni tikamache pali nzeru pamenepo umenewo ndiye uchinderewo

 3. kaya mususa,koma ndakunena zoona malawi wake yemweyi madzi ake omwewa,mages ake omwewa,atangobwera azungu ndiulamuliro wawo madzi sangamasowe,chakudya angamazilimile chokwanira,magesiso sangazimezime,po ife timatha ndikuyamikila mtsogoleri ngakhale akugona,ukuyesera kumuzusa akuophyeze kanako timanganepo then ena aziombera mmanja mmalo molimvera chison ziko kanthuli,till now adamac sinasegule misika anthu akuvutika kut apeze chimanga ,ndewina akadandaula bas mummunge,Mlungu pulumusan malawi kumavutowa coz ndikwainu nokha komwe sitingamangidwe koma kupasidwa zomwe tipempha komaso muwakhulukile onse akuchitira amzawo zoipa mnmnga ifeso tawakhulukila mangawa anthu,mut pase maso auzimu kut tione patali ngat mene aonela enawo,pamene mukudalisa maiko ena ifeso amalawi mutidalise komaso mutiphumzise mtima wakuyamika.

 4. Amalawinso pena tikuonjeza tanyanya kuchulukana iiiiiiiii nkhani yake kudalira makala basi.
  Madzi okanganira,Magetsi okanganira,Ntchito yokanganira,Zakudya zokanganira,Mowa okanganira bolako mwina akazi ndiosakanganila nkhani yake tanyanya kuchulukana dziko lachepa ili ndiye tisamangoti boma,boma,boma kodi nanga ife tikuthandizapo chiyani??????Maiko olemera ambiri chiwerengero chawo ndichochepa kwambiri poyerekeza ndidziko lathuli for example Botswana tafufuzani.
  Koma ife aMalawi kuswana ngati mbewa basi ndiye mkumangolimbilana tizinthu tathu tochepati.

 5. So we shld say that we(malawian)have the right tu xpress our opion over govt matters?.We must also oppose where the govt is failing,and it is the responsibility of the govt itself to ensure that the wellfare of it citizens,is condunsive/being improved both rural and urban area.So i can say that the govt shld focus on issues which can achieve/promote development on our country.And may God bless malawi.

 6. Iwe Billy ndi muthu wa a degre ndipo osati imodzi protest nkoyamba anayamba ndi bakiri bingu wazipeza tazingodyani kfcyo mukanakhala anthu b wezi muri kumalawiko kuthandizana koma muri kuno chimodzi mmodzi ndimasavage ife ndiye khalani pheeee olo kunmangako fusani sikoyamba koma siku rina mayaya mulungu anzamuthandiza malawi nkuzapenya

 7. MALAWI IS FULL OF DEAD PPLE YES WE A ALL ZOMBIES I MEAN IT .INU MAGETSI ALL OVER AKUXIMA NGAT DOSAGE YAMAKHWALA MAMMAWA,MASANA ,MADZULO NDE MUZITI WINA TO VOICE OUT WALAKWISA IFE TONSE TILI PHEEE ET. MUYAYA WAS FIGHTIN FO US ALL AAAAAHHH WE BETTER JUST SELL THIS COUNTRY BAS ZATIKANIKA AMALAWI .AS FOR ME AM NW REGRETING FO BEEN BORN HERE .

 8. But police y? Insted of aresting the minister hu showd hiz Tumbukan big blak un circumusized penis in public y aresting some1 huz fighiting for our change?

  1. For you to say tumbukan uncircurmcised d… …, mwalakwisatu, paja abale anufe ndifeso atumbukatu, maybe am looking at you the wrong way all along, are you a triabalist?

 9. Misonkho timalipila magetsi madzi njee.Tsono mwapangazo mwapanga ngat ana chifukwa zionetsero zomwe takonza sizamtendere,zipangisa wina yemwe akudwala bp ikwere mpaka 330

 10. chikuvuta kwambili kwathu kuno ku malawi ndi mantha chilungamo timachibisa kamba koopa chitukuko chikufa kamba ka mavuto a zandale blakout/water shortage plus more zikubweretsa mavuto akulu kumtundu wa amalawi katundu oyenera refrigreting akungoola kamba ka blakout sizabwino zigayo allwez off chonde amalawi tisagone ufulu wathu usamphanyidwe mwanjila ina iliyose tipange chimodzi tikweze malawi.

 11. But then demo for who?i felt escom claims low water levels for the problem?after demo,power was to be restored right away??amayaya zanu izoooo.

 12. Muku nyoza mayaya coz kwan wina sana ferepo pa oxygen bola uzakhale iweyo.Apolisiwo a DPP akugona mu mdima kupita ku vep osasa kom kumanga munthu.Yes bwana ameneyu mupenga nazo

 13. Unbelievable! Just let the man walk! The Police has lost direction! Or maybe the police is also another youth wing of DPP?
  I thought the blackout affects all, including the police!

 14. Apolice amamufuna kale ndi kale mayaya bcoz iyi singakhala nkhani yomumangira. anthu akufa mzipatala?biznez za ima.kodi chitukuko kumalawi chibwela bwanji ngati magetsi akukanika kuyaka?zopusa basi

 15. Apolice ngati simuziwa ntchito siyani ntchito amaba,kapena kuonesa kusasangalala ndizomwe zikuchitika? Shame on u malawi police osamanga njala bwanji umbuli winawu

 16. Amtulutse ameneyo azathu kuno ku SA akafuna magets kapena manyumba ama RDP amapanga ma Demo kt boma liwathandize mwamsanga .Ndinena pano zinachika mwez wa Jun .16 ,2016.Chonde2 Mtulutsen aboma!!”

 17. kupusa nthawi yamai magetsi amayaka bwinobwino,madzi samavuta koma Ankolo zimenez zikuwavuta chifukwa chan? Agalu inu a DPP chitengelen boma palibe cholozeka chomwe mwapanga,msaname Mai Joice Banda tikuwadandaula

 18. let him lot in the prison. what kind of humanbeing is he? water level is low and he is protesting for what.? he must protest to heaven if he want contineous water levels for contineous electricity. foolish man arrest his friends as well.

 19. its only in Malawi where a majority of cowards want someone brave to fight for their freedom and the best they can do is just sitting mphwiiii!! commenting on a Facebook post throughout the Day….Where I come from people talk on the streets & not on Social Media ….

 20. Hello friends, my name is Esther Mashabai was one of those millions of people living with HIV/AIDS, i received my breakthrough with the help of Doctor Abumen whom i met through the testimony of someone he has helped, after some series of conversation with the person sharing the testimony i decided to contact Doctor Abumen which i did, after some negotiation he sent me the medicine with an instruction on how to use it, i notice some change in my body when using the medicine, after completing the dose as instruct i went for test only to be confirm negative by the doctor after the result came out, words on the internet can not express it all, if you are in the same condition and you are looking for a way out of it you can contact DR ABUMEN on his email address,([email protected]), or you can call or whatsapp via +2347085071418

 21. we dont have human rights activists in Malawi all we have are fortune sickers thats why they are not stable .They can move in any direction where the wind blows as long s they get what they want. I cant sympathise with these people because they have let us down due to there greed.

 22. Remember Its Towards Power All Day not Power All Day Ndye Escom Itha Kukhala Yolakwa Kwa Anthu Amene Muli Ndi Ma Bznex O User Ma Gex And Too Escom Itha Kukhala Yosalakwa Kwa Anthu Amene Mulibe Ma Bznex O User Electricity Or Ndnu Olembedwa Kmano Kt Tiyangane Balizose Escom Itha Kupezeka Yolakwa Why Cause They Promised To Give There Best And Kt Muone Sakukwanilisa Kt Muwafuse Akuuzani Kt Ndalama Zambil Zmapta Ku Chpan Cholamula Kupangila Kampen Kt Boma Libweze Czmatheka Ndye Pofuna Kukonza Muyambile Kulikulu Then Kumatsika Musimo Zmenez Zingatheke Pokhapokha Ma Bungwe Atalowelelapo Apo Biii Tizingomangidwa

 23. Mwamangilanji munthu otimenyela ufulu komanso sanatenge cida kusiya kukasaka mwana waci albino wasowa kusukuluyo apa zaziiiiii ati a polisi mucite timanyumba ngati makicheni

 24. Kodi pazinthu zimene sizikuyenda bwino kwa ife ngati eni nthaka,Manyasa, kapena kuti Amalawi tikuyenera kutani kuti Boma lidziwe? Kodi tikuyenera kuwopa kunena chilungamo? Anzathu andalewa amatifuna ife mnthawi ya chisankho koma akangosankhidwa ife timakhala ngati dzikoli silathu, kodi ndi chifukwa chiani amapanga zoterezi m’malo mokonza mavutowa?

 25. Nde Mmene Ammangomo Magetsi Akuyaka Ndinso Madzi Akutuluka? Mukanaona Kaye Mfundo Zake Kenaka Action, Apa Mukutanthauza Kuti Zinthu Zili Bwino, Koma Mmene Munganenere ( Climate Change ) Isovedwa. Nde Tingokhalira Climate Change Nde Tizingovutikavutika Nkumandaula Za Magetsi Ndi Madzi, Zukutani, Ongolerani, Kambani, Zoti Zitidatse Ndiponso A Malawi Asangalale Nazo

 26. everyone knows the problems shortlisted even the government thus BILLY MAYAYA could suggest solutions to those problems because he too is a victim. demostrations do not solve problems instead resources are plundered

 27. Kulaka laka kuthawila ku mozambique
  Komano nakonso kuli nkhono kayano nkumatani

  Kunene chilungamo boma kamalawi pano likupweteka mmitima mwathumu
  Nkhanza kuchita kuposa idi amini

 28. So we are back to the tym ov police align with gvment arent they feel the heat whn a coutry gt no power fo 2dayz yet the power supply insist to hike the lates ov it while we dont hv such supply? Anyway no supprise as even his brthers admistration does the same to manupulate the police office

 29. Mr Billy kupanga zionetsero sanalakwitse malingana ndi mavuto omwe a malawi akukumana nawo, koma anayenera kutsata ndondomeko yake, ndi chilolezo cha a police, tizitengera phunziro kwa anzathu a ku R S A, apolice amakhala patsogo enanso pambuyo pa anthu amene akupanga zionetsero ndipo a police kumangokhala kulakwa kuthamangitsa anthu, iwo ntchito yawo kuteteza anthu amene akupanga zionetsero

 30. Amalawi sazatheka to hell with anything here leave non African way of life and fallow our on coz izidzikuchitika chifukwa chaumbuli kumatsatira chilichonse chakunja

 31. As a country well known to be full of peacefully citizens this is one among many umwelcomed developments as such there’s no way in resorting to violence so as to gain attention and neither is arresting those trying to demonstrate over issues of blackouts among others a solution.

 32. we all can see that zinthu zativuta tonse and its not the government which is switching off the electricity deliberately. We all know the probldm of global warming has brought disasters such as drought which has led to Malawi having these problems we have. So where is wisdom for someone who went to school to go and demostrate aginst the government for such things as if its Muthalika who is doing these things?????? why not demostrating against those who are contributing to global warming in large ammounts???? u deserve an arrest for sure coz thats nonsese but just to bring BREACH OF PEACE

  1. are zambians,tanzanians, mozambicans experiencing the same Blackouts problem ? Hadnt been 577bn Dpp cashgate malawi would have bought Power from mozambique.Would have processed charcoal to generate electricity.,a clever leader would have wooed investors to establish Solar electricity,But alas !! malawi is run by Thieves and Liars.

  2. muwauze abale anu omwe ali phepetele mwa mtsinje wa shire asiye kudula mitengo mwachisawawa dont blame mr president he is not the one who is destroyed the trees shame on u people

  3. Koma Ndawerenga ma comments ambiri pa page yi, ndaona kuti amalawi ambiri tili mdziko lino koma sitidziwa zochitika mdziko lathu lomwe…Ku south Africa Over 50% Ya magetsi awo amachoka ku mozambique, The late Bingu said that lets have interconnection from mozambique by then some amount of money could be funded by African Development Bank,unfortunately the parliament denied that Bill claimed that its expensive…i really dont understand mpaka pano why they did that..He bought another hydro-power of which dr Banda launched..but we still need some more electric power supply…now this govt came imayenera ipitirize kusova…koma ndikukuza last week zodiak idacheza ndi avice president achilima pa za nkhani za magesi,,A VP adati plan yawo ndiyoti akufuna kugawa escom board pawiri..Ena adzipanga magesi,Ena adzigulisa..mtolankhani adafunsa kuti zimenezi zithandiza a VP adati Eya.
   Now ine ndidazizidwa nkuganizira mmene zingasinthire ndiye mwina inu mukhoza kuganiza mozama bwino za mfundo koma ine ndikukanika…PEOPLE MUZIZITSATA ZINTHU POMVETSELAKO PA RADIO ANTHU AKAMAFOTOKOZA, Ndiye muzazimvetsa zinthu maganizo anu azikhala mmalawi muno dont think outside the box..AZIBALE AKUMWALIRA CHIFUKWA CHAKUTHIMA KWA MAGETSI..Iwowo ali kuchipatala sangathe kudzimenyera okha ufulu wawo koma ife amene tili olimba..u know anthu amamenyera ufulu wa anthu osati wa mbadwa inu okha koma wa ana awo (other generation to come)

  4. Mathew i like ur intellectual u seem to be well informed but, even if we go to the streets what will change?? anthu akangoswako ma shop basi??? kuonjezeranso mavuto ena?

  5. wake up Malawi escom shud not fool us it’s not about water levels BT politics has engulfed escom madzi ayamba kutsika lero?. … enanu mumapereka makomenti opusa ngati zonse ziri bwino kwa inu. … shame on u

  6. mbuzi ya munthu iwe mbuli yophunzira global warming ili kwanthu kuno kokha bwanji maiko enao kulibe zimene zili kuno Mulungu atikuonzera mavuto athu amwalire basi watikwana

  7. global warming? can we say that global warming has just affected Malawi? why the neaghbouring countries not experiencing de same problemz? zausilu bas ma black out ati kwana

  8. The idiots say “chisinthe ndi chani” educated pple forcast then they find the alternatives b4 its too late. In malawi the prebians are more educated than the government itself ie they buy gen sets in time of black outs

  9. Malawi is nt independent yet en we need our leaders to bail us out frm dependent. If we need donors to support us wit de projects of pumping water frm de lake to lilongwe, solar power, coal energy,funds for butimen roads across de nation etc. US, Britain,Canada,UAE,China, Japan, Germany etc also need our support nt them to support us always

 33. Some of us are really stupid.. This fool uses demos to get funding from abroad.. the fact that his friend Mabvuto Bamusi is now presidential advisor, he is confused and disappointed. He wish he could be the one… This stupid idiot is telling pple to match with Chacoal intheir hands yet it is charcoal production which has led to the shire river to be full of siltation… this idiot deserve to Rot in jail…. WE NEED SOLUTIONS AND NOT PROVOCATIONS AND DEMOS,,,,STUPID

 34. Kodi amalawi mumaona kuti mavuto angathe ndi maemo? Sindiye kupepelako kumeneko, mukakayenda panseu ndarama yokonzera magetsi muyipeza? Amuchitabwino wakulawako

 35. achichita bwino…mesa anakayamba kupeleka altnative way yothesela vuto lamages nd madz..akapanga ma demo ndekut madz azpezeka mmisinje? kmaso asadandaule jail is th destination of evryman..ma freedom fightr anakwana kale..malcom x and my frnd tupac. enawa ndongofuna kukhala mu history ya malawi opanda chanzeru chochta ngat achna lodney king

  1. iwe ndmbuzi yamano kusi mose boma linayambra tkufuna njra zothetsera mavutowa mpaka 2yrs nde udzthoka mbwerera zakozo mbuzi

  2. Dont u knw ntchito ya minister board chair ma engineer?Ndiye zipanga seek nzeru kwa ife?Umbuli ukuvutan.Tiwauza kangat akukanika kugula ma battery asoral pa KIA mapanel awulele so what do u expect from us?Mot nzeru ulibe pamodzi ndi anzakowo?

 36. Nthawi ya Bingu wa Mutharika kunkapanganso ma Demo nthawi ya Joyce Banda kunkapanga ma Demo lero ndi nthawi ya Peter ma demo mukupangabe tsopano inuyo a Billy Mayaya ma Demo mudzasiya liti?

 37. Bwana Bright! Zomwe anthu amakambirana ku parliament kuja zimakhaka zokomera okha. Nanga ife omwe timawavoterafe amatifunsa maganizo athu ngati? Ife timangomva zothaitha kuti akuti agwirizana zakutizakuti. Ife mmatifuna nthawi yovota basi koma mukawina ife timakhalano agalu! Ndiye polankhula muziyamba mwaunikira kaye kuti kodi amzanga akumva kuwawa bwanji umoyowu chifukwa mwina mkutheka inu za mavuto mungomva anthu!

 38. mwamuchita bwino, mphamvu zamagetsi zomwe zilipo sizingakwanile kukhala ndi magetsi madela onse nthawi zonse. bwanji osakayenda chifukwa cha anthu amene akuwononga mitengo? moti iye sakumvetsa chomwe chikupangitsa kuti magetsi azime? nthawi zonse ndimakhala kumbuyo kwanu koma lero lokha ndiye ndi uchitsiru weniweni wagalu mwapanga apawu.

 39. Asa!! U Police Officers Why Arresting Billy Mayaya, Don’t U See That We Malawians Are Suffering Cauz Of Blackouts? Escom Why? The Moment Iam Speaking Here There Is No Electricity, So U Police Officers Ur Favouring Escom For Doing This Nosense? Day Before Yersterday Ur Fellow Officers Arrested Two Security Guards For Beating & Killing Athief In Thyolo Instead Of U Thanking Them For Minimising Thefty U Arrested Them Why Police? Today U Arresing Billy Mayaya For Fighting Against Blackouts & Shortages Of Water Lack Of Proffetionalism From Police Officers, Please Police Stop This.

 40. Malawian police so stupid. Do they have electricity in their houses throughout? Iwowo sawonapo vuto?We are going backwards as a nation

 41. Amuchitabwino kape uyuuuuu!!!
  He always criticise each and any Government, he has no crew what is looking for.. He was the first guy supporting APM and DPP, he criticise JB of being a bad leader and now what the f**k is he complaining? Muchimange kwambiri chi idiot!!!!

  1. Man inuyo palibe chomwe mukudzi mwina simuli ku malawi kuno kwa miyezi itatu magetsi osayaka masana ndizabwino zimenezi ndiye anthu kukafunsa alakwitsa? nkhanitu siyazipani ayi koma boma ndi anthu ake.

  2. Man, mwina sukundimvetsa bwino…
   Am not supporting government, first it is very bad for citizen living without water and power.. Nobody can be happy with the situation going on in our country..
   My point was just for this guy you call him Mayaya, he was in UK few years a go talking too much about JB that she was not strong enough to be a president, better APM he has a great future… So now what is he want? The same guy who he was thinking that has a great future now he is trying to get this country to a mess…
   It’s good that he complain but I don’t like he’s idea as a freedom fighter, he is totally filed.. He don’t know what is looking for, at the end amwalila imfa yowawa

  3. Kulibwino amwalire Imfa yowawa koma azuzula,,,,,Listen brothers,,,;,,,,ucan support DPP mean whiel ngati yikupanga zopusa DDP aliso ndi mphamvu ngat citizen,,,,no mater ankasapota DDP,,,koma pano zafika wesi or ineso ndikasapota DPP koma pano nde IBu wandiskasa bwanji,,,,Ndikabwela ine ndizapangaso zina kamalawiko Ndikochepa sikangandivute,,,,,ndimaopa Mulungu osati Apolice ndi Ibu,,,Bily Mayaya ndakuyamikila ilike ur Brave.

  4. Kulibwino amwalire Imfa yowawa koma azuzula,,,,,Listen brothers,,,;,,,,ucan support DPP mean whiel ngati yikupanga zopusa DDP aliso ndi mphamvu ngat citizen,,,,no mater ankasapota DDP,,,koma pano zafika wesi or ineso ndikasapota DPP koma pano nde IBu wandiskasa bwanji,,,,Ndikabwela ine ndizapangaso zina kamalawiko Ndikochepa sikangandivute,,,,,ndimaopa Mulungu osati Apolice ndi Ibu,,,Bily Mayaya ndakuyamikila ilike ur Brave.

  5. Bombokrate man!!!! Black out its been there since Bakili Muluzi!!
   Talk about economy isn’t good!! That bombokrate Mawaya is nothing but trying to be famous.
   Tell your government to resign, m’mesa munkati amayi JB sakuyenela kulamulila dziko? Nde lero mukulila chani? Munya simunati…

  6. Aaaaa i don’t know what this guy tries to think!! Of course blackouts were there during Muluzi,but a normal person cannot go in the streets saying am having demostration meaning obstacles of Achewa mmmmm Amigo this is 2016 let us do for current Leader.

 42. Mayaya sanalakwe sibwino nthawi zonse kumangokhala chete kulibwino kuchitapo kanthu mavuto ambiriwa kwinanso ndi kusowa ndi kuzimazima kwa magetsi chonde tachitaniponi kanthu Malawi apa ndiye akubwerera pambuyo magetsi madzi munthu ndiye atani ndikhondo imeneyi dzisankho mkumabera kuyendetsa dziko ndi ai koma kubomako muphana anthu inu

 43. Mayaya is an innocent man,coz these blackouts bring dealth 2 our beloved relatives in hospitals e.g operation,oxygen etc hw can it wrk wtout electr..& 4 water..eh brethren worse than b4.Mind u,water iz lyf

 44. Bwanji osagalamuka malawi! Madzi akhalepo asakhalepo magetsi amadzima monyasa mwezi siumatha magetsi asanamizimepo,mmalo mogula zipangizo zatsopano zamagetsi zowonjezera mphamvu,kumangogwiritsa ntchito zaJohn chilembwebe mpaka lero,aaaaaaaaa Malawi! Koma kunjika ndalama mmanyumba mwanu ndi kukabanka mayiko ena basi, zithandiza chani mtundu wa amphawi owophsya padziko lonse lapansi,Malawi chomwe akudzi ankatangale koma opandanayenso phindu.

 45. Amangodzuka mamawa basi ali ndikupita kukachita ziwonetsero opanda kudziwitsa a police ndi a city council? Makani enawa mapeto ake ndi amenewa. Mutsekereni tikamuchita bailout next week mpata ukapedzeka.

 46. He is one of the man we want in this shameless country Malawi,Billy we our on your side, strong people like you its what we want not coward people. Dzuka Malawi chotsa nkhungu zosakutherazo.

 47. Malawi sinzachangamuka ths why zikatiwawa tmangobuulila mmimba chomwew timaopa ndikuoswezedwa komaso ingakhale kumangidwa kumene,mmese mumati kuli democracy,komaso ufulu wochita chithu posamphwanyila ufulu waena? Kodi wamphwanja ufulu wandani mwamumangayu?malawi nzuka,nzuka malawi nzuka kutulo tomwe uli nato.

 48. komaso vuto ndiloti amangolemba apolice ka kampira ma results ake ndi amenewa komano boma lathu kaya likupita kut y kamudzu u left us earlier

 49. Eee achita bwino iyeyo akufuna kuchuka pofuna kugwilisa ntchito athu osauka,mmm nanga bwanji osapanga mphavu zamagesi bwanji? Mazi apwela ndiye iyeyo agwese vula lelo popano ngati ali wazelu.

 50. If ma DEMO could change things for better, then the worst things wouldn’t have happened pa 20 July which is my birthday.
  Something nasty was added on my birthday coz of these POLICE n BOMBO CRATS POLI_T_SHIAZ!!!!!!! Informers manonga me yard tryna blast dem yut pan d street ffi dweet a likkle som’ ffi de betterness ffi we contri!!!!!

  Once again BOOOOOOMBO CRAAAT TING to Malawi24!!!!

 51. It’s just the same thing in our country called Zambia. There are special pipo whom they can not be arrested even they do wrong things but others they are arrested even if they are doing right thing.

 52. Therez no way pple have to ask these stupid police to stage demonstration bcoz u wil not allow to do so. Police always save the govt of the day, of which r part n parcel ov de same shit. There4 its our own resposibility to speak out our grievances thru demonstrations without any intimidation from unprofessional police. Thank u

 53. I THINK THE ARREST IS A POLITICAL VENDETTA AGAINST THE DEMONSTRATORS AND AN IMPINGEMENT TO HUMAN RIGHTS. I DO NOT SEE ANY CHARGE LEVELED AGAINST HIM AS AN EXPERT IN HUMAN RIGHTS LAWS. POLICE ARE ACTING OUT OF IGNORANCE AND STUPIDITY. LET HIM BE FREE. THE COURT THAT WILL TRY TO FIND A CASE FOR HIM WILL JUST INCOMPETENCE AND LACK OF PROFESSIONALISM. POLICE PLEASE BE PROFESSIONAL. NYUMBA ZANU MULIBE MAGESI NDIYE ANTHU AKUFUNA KUKUMENYERANI UFULU MUKUWAMANGANSO. MUSATIKUMBUTSE KU EGUPUTO A MYP.

 54. olo mutabwelesa boma lina palibe chomwe chingasinthe! kodi magetsi ndi madzi zinayamba liti kuvuta? inuyo ngati okhudzidwa mukupanga chan? zimaoneka zosangalatsa ku parliament kuja aphungu otsutsa akalephela kuvomeleza kanthu kosavuta monga kutenga magetsi ku mozambik! kodi nthawi imene anthuwa anakana zimene zija bwenzi pano magetsi akuvuta? lelo lino bwb likufuna lidzitenga madzi ena kuchokela ku likhubula mphili la mulanje anthu ena ati ayi,muli mizimu ya makolo awo! ndie mukut chan? amangidwe basi amafuna kuyambitsa chisokonezo anthu akaba then apolisi nkuwaombela omwewa ma activistwa azafuna boma liwapange compansate mabanja anthu akubawo! instead of kugula mankhwala mzipatalamu! zautsilu!

  1. Iwe ndimbuzi!ndiuze boma lomwe magetsi anavuta ngati lilipoli.Uzachita manyazi ena atabwera ndikukonza zinthu. Ukumbukire mmene mafuta anavutira but it was done just overnight by JB.

 55. Only dpp khadethisi blame Mayaya,does this government want people to suffer in silence? When we talk they arrest us,God is not man so wait and see that left hand will also paralyse.Ndatukwana ngati….

  1. Mayaya spent a night in police custody which is very painful to some of us,yet you are quiet.Just because i talked about your father there you now talk.To hell with your nonsense ok

 56. Demo is not a crime,its therefore,a crime if you do it without proper procedures….aMalawi,tiziona chatsitsa dzaye,osamangoti,dzaye latchola nyanga ya njobvu

 57. mwamumanga chifukwa chani agalu inu….ndiye kuti kudzimadzima kwa magetsi ndikuvutavuta kwa madzi zikukusangalatsani eti anyapapi inu?????…zauchitsiru basi…kuno ku blantyre simunakayelekezeza kupanga manyi anuwo…ifenso kuno timatcha …..bwanji osazimitsa magetsi komanso kutseka madzi kwa one week kunyumba kwa president aone momwe zimapwetekela?????????????

 58. aa apolice akumalawi mbuzi bomalathu mbuzi tsogoleli mbuzi a dpp mbuzi mwalomomanga matenda womwe akumuvutitsa tsogoleli kumamanga munthuwoti adandawulila amalawi kunkhanizamagesi zowona ndinu mbuzi nose ndinu mbuzi

  1. Inunso man ndiye mbuzi yoheratu mukuyesa Mayaya wanuyo akapanga mademo magetsi abwera.Malomokhala pansi nkukambirana koma munsewu fotseki ulendo wake uno kupanga zopusa akumangan kwambiri nayenso mutu wake sukuyenda ndimomwe munamunamizila kuti wafa.Sanafe mulungu akumumenyera nkhondo nkulu wakenso amubweza kuti ayi dikilira kaye umalize term yako 10 yrs

  2. ukunama kuti anakambiranapo ku malawiko zithukusitha pakutidziko lilimanja mwagulu ine ndimati alipire mbuzi ndiye iweso majemaje ulikufunika mbuzi safa inesindimafuna kuti afe ayikomapakutiwatelo kusalakhula komwesakulakhulako ngatimbuzi sachira afa siwabwereraso kuchipatara uwona Decembar safi ka udzandifuse udziwachani iwe ine ndikudziwakuposayiwe

 59. Akanatsata njila yoyenela ndikupatsidya chilolezo chopangila demo..koma chomchi ndy ndiudyo…koma amafunila kupangilazo ndizoveka..magetsi,madzi zafika pa worse…koma apanga puma…

 60. Y Malawians owez huv low self-esteem ?? Malawians wake up!!!!,no time 2 slip!!! du yu think zin2 zingasinthe without your efforts?? Maiko anzathu amapanga Ma demo just becoz magesi azima kwa 6hours SA iz an example for that matter…. why Malawians???? sizikukuwawani??? magesi kuzima morning 3 oclock morning kuyaka mid nait mun2 ukugona, upita nthawi yanji kuchigayo??? how about welders can they du there job to support there families financially??? Malawians why??? zaka zonsezi madzi amasowa 2004 iz a very gud example but magesi sana3ke apa?? Malawians su you think Escom ikayasa magesi madzi amakhala abweleramo mu ma responsible riversmo??? y blaming #mayaya Malawians ye he oz fighting f

  1. thus fact tangoganizani mu2 akudalira bershop kt adye komaso pali ana akudalira iyeyo magetsi chizimireni chadzilo do u think adyetsa ana or lent alipira gyz zinanazi tamaganizani kd ndi ma blackouts ake amenewa mndani angaganize zodzaika factory yake kuno kumalawi tangogani iweyo ukuzitcha mmalawiwe tapita misikamu okaone mmabutcher ngat zinthu zikuyenda nde ukamve fungo likutuluka mmenemo gyz humanity ndiyofunika kwambiri iwe uterowe ulindi Genset panyumba pako kwaiwe zingathe kukhara mnkhambakamwa chabe kma uganizileso moyo wamzako kt magetsi kulibe apita bwanji kuchigayo mulungu akuoneni mukulankhura ngat madolonu shame on u!

  2. my fellow malawians we hv to work up so that we cn fight for our freedom of express,lets join hands 2gether so that we should enjoy democracy.am depending on barbershop as my business but magesi akumazima 3am and akumayaka @ 11pm ,then my question is what time am going to do my business

  3. demonstrations is a constitutional right but the procedures must be followed of which Mr Mayaya did not!!! umbuli uwu mukukamba apawu

  4. Hurry ukunama, zinazi mutamaona kaye, izizi zikukhudza aliyense even munthu amene sakhala nyumba ya magetsi ku nkhani yaku chingayo ndiponso ma procedure ukunenawo ndi ati? Aja amati mimseu bweee aja anatenga chilorezo?

  5. #Hurry du u think ife or mayaya sitinapite ku xul?? sukudziwa kuti some procedures are not to be followed?? we r suffering now kut tiyambe za procedure ukuganiza ngati ma Demowo adzachitika chaka chiti?? dont u av wisdom?? zoti kusata all the procedures ma Demo sangakhaleko ukudziwa??? i think u need to define the term “” DEMONSTRATION”” u can even sic 4 assistance if needed…. ma demo mun2 samapanga akukukondwa…

  6. koma abale anthu enawa mmutu muli madzi zoona magesi ndi madzi mmene akuvutiramu nde kukabakira boma kuti achita bwino kummanga #Mayaya pamene munthuyu amafuna kukhoza zinthu. woke up malawi don’t be like a dog sleeping during the day” akasaka liti? well spoken #T_Captain we’re behind u bro

  7. Ndondoneko???? Mr Billy planned this yesterday, ine ndidamva paZodiak kuti mmawa akapereka petition kwa dc kuti apange demostrate pa za vuto la madzi ndi magesi

   Ndiye pali ndondomeko ina???

  8. Petition kwa DC kuti apange demo? iye amakapanga ma demo asanapemphe chilolezo ku Police, ndi ku City council that’s why amumanga, akanamupambazanso makofi

  9. By the way the constition does not say you should seek authorisation ,Rather you just give a petition to the DC and the DC through the police shall provide the security to the demonstrators

   The republic constitution Section 38.Freedom of Assembly Every person shall have the rivht to assemble and demonstrate with others peacefully and unarmed

  10. zaSA wanama m’bale since Sunday magetsi akhala akuvuta kuno n no one went on the road or to municipality for demos, osamawanamiza amalawi apa, iyaaah, moti dzana Sunday sitinadye usiku even dzulonso

  11. Komanso anawuzidwa kuti asinthe siku koma iye anapanga makani, amvekere come rain come hell ine ndipanga, achita bwino kumumanga

  12. Kukhalalila Back Boma,,,,,pamene ana ama minister akugeya anyezi kamba ka Vote Lanu,,,,,,,,,,,,,,Congratulations to Billy Mayaya,,,,,as am a Pastor iwl curse to all Police those who arrest#Mayaya..God should punish them like He did Byblon,,,.MALAWI MUKADALIBE KUDYA madeya.

  13. Zoona magetsi amazima sitikukana,koma panopa awonjeza kunena chilungamo,madzinso chimodzi modzi,ndiye maka maka m’makwarara momwe ife tikukhara nanji,dziko lathuli iiiiii pemphero likufunika ndithu,tsono zomatchazo maiko anzathu zimatheka ndithu zantendere bwino bwino,koma mukayambanso kumanga anthu ndipamene anthu amalusa,kenako athu osalakwa amafa zidza.

  14. Ndichifukwa mayayA amayeeesa koma nomwenu umafunila zoyipa m ukuwona ngati mayaya made no wayamba zulo sakuzuwa kopita vuto ndirimenelo a malawi mumatengedwA kupusa ndichifukwa zithu akuchitilani mmaso nwanu m malo mokufusani poti nonse zisilu akusakhilani erectro comision wina opanda kukambilana ku parliament azabereso chifukw ndinu mbuzi kuti wina akuyimmileni bwebwebwe bola ndikanabadwila ziko Lina osati nyasaland mwazaza educative survages

  15. Palibe chomumangira munthu apa thats why mr president is sick coz of nkhanza blv u me malawians wl experience hardtimes this coming month &ofika 2017 ayi ndi mamuna

  16. C hisanzo kuno kupanda toys toyi Zuma b wezi akutubwa mpaka pati koma poti anthu anasegula mmaso relo akuziwaso kuti phAvu ziri ku wathu osati kwamata chipere ndikumapanga zofuna zawo muzaxuka riti MalaWi

 61. What permission is the police looking for? Did Escom get permission for Black out ? If yes from whom and why people are complaining now ? It doesnt make sound wake up Malawi

 62. Ndakatulo ya mbuzi,,,, adakaionjezera kaah, womanga amademo mbuzi
  , wochita mademo opanda zikalata mbuzi, komaso wokaniza makalata akudemo mbuziso, Amalawi lero tikukonda mbuzi # CHIWAMBA #

 63. Chosecho amene akugwilayo nayenso kwawo kulibe magetsi ndi madzi omwe! Akaweluka akafunsa akazi ake ngati madzi akutuluka or ngati magetsi akuyaka! Shame!!!

 64. Koma munthu sumangozuka kuti lero ndikukapanga ma demo, amalawi tiyeni tiphunzire kusata chilungamo. Ploice always discharge its duties but only get insulted as the rewards. its against the role to juat demonstrate without seeking permission.

  1. By the way. The Constitution doesn’t say you should seek authorisation. Rather you just give a notice to the DC and it is the DC through Police who shall provide security to Demonstrators. The Republic Constitution says in section 36. Freedom of Assembly Every person shall have the right to assemble and demonstrate with others peacefully and unarmed.

  2. iwe sankhani ndiwe chitsilu galu zoba munthu wazelu sungakapempheso chilolezo azibale athu akuvutika ndiwewakutchyolo mbuli zachabechabe u profesawo ndiwumanewo ndiwechitsilu tidakakomana pamasompamaso ndidakuvaka mbama ndimadana ndianthu akula mopusa

  3. @Nanthambwe, you have never heard of police or DC telling demonstrators that they should not demonstrate for security reasons? That means they are not allowed to do so. I think we over understand democracy. Democracy without responsibility is nothing. Democracy doesnt end on you, it extends to others as well

  4. chimbalanga you will hold your own demostration tommorrow upon seeing your son or daughter dying on the life supporting maching….am not in Malawi but u r the only creature smiling may God punish you 10%….for you to face the cryo of the Nation alone

  5. @Columbus, every malawian is very concerned with the state of our electricity and am not happy too because my business has also been affected. The issue here is that, the guy Billy Mayaya amapanga zinthu ngati saziwa choyenera kuchita at a time. Its not first time for him to demonstrate but the issue is procedure and nothing else. The issue you are saying that God should punish me and all the evil wishes you have casted on me, I declare in the name of Jesus Christ of Nazareth, BACK TO SENDER COLUMBUS EMENACE

  6. Billy Mayaya as an activist he knows very well what to do and what procedures he should follow when staging demonstrations, so lets not blame somebody here, he himself is the one to blame period.

  7. kutsata procedure yopanga coment pa FB si udolo. anthu mumangolankhula inu hypocrites that’s y you sit here and let malamulo get screwed uo

  8. Iwe #Sankhani tandiyankhe funso langali» kodi vuto lamagetsi ndimadzili kwanuko kulibe? or mwina ukukhala kumamidzi koti magetsi kulibe ndichifukwa chake ukuyankhula ngati mwana wakhanda; dzuka m’bale wanga usagone

  9. kkkkk eti eti iwowo apangapo chani monga mmodzi wa anthu okhudzidwa? kupusa mkulankhulatu uku ,konda dziko lako la malawi pozindikira kuti likukumana mavuto ,njala mavuto azachuma matenda nsanje ,nanga mungatiuze chomene chikuzimisazimisa magetsiwo ayi simunganene koma kutukwana,,so,,sometyms ma activiswa muziwamva kaya sound b4 surpot them ,,pepani sikuti mutukwanetu apa,,

  10. The Law Doesn’t Require Police Approval For A Demonstration, Only To Be Notified!!! Our Stupid Police Should Enforce Existing Laws Not Imagination!!! I Feel Sad That The British Wasted Resources In Reforming These Brutes!!!

  11. Nde iweyo ukuonakuti ndzabwino zmene apanga apolice’wo?? Schifukwachokwanilachmenecho iwe kulianthu anaba ma billion aja osakamangaameneajabwanji?? Iwe nde ukusekelelankukamwazopusazo kambeu kaanthu ngat inu ofunikakukakaponyapamoto zachamba kaya unakhalilanji mzanga pa fb aaaaish!!!!!!!!

 65. Paja Mumadana Ndichirungamo Apolice Ndinuzisiru Kuzorowera Kurowa Zokumba Eti Ndikumwa Mazi Amuzithaphwi Munyumba Mumaunikira Koroboyi Ndikuphikira Zachibuku

  1. Mmmmm! Mr j tambala bodza ilo inu pamalawi pano munthu kupanga chilungamo zimaveka palibe zimenezo wanga chilungamo anthu ambiri matsiku ano akugona ndi njala chifukwa chamagetsi sure mmmmm is to much now anthu atopa

  1. kkkkk I was just asking, public demos always take place unless government or court offer permission to do so, if not that’s is always a case as constitution says. if he was not granted permission to do so, he will face law cos no one is above the law

  1. Achimwene popularity means not ur on top of laws. I,m affected by blackout aliyense m,malawi muno knows the situation we r in ku nkhani za magetsi. Koma any demonstration pamafunika chilolezo ok.

  2. Anthu inu muziganiza polankhu mu2 nditsogoleli wa bungwe limodzi lofunika mmalawi muno kma z alawyer akudziwa malamu adziko momwe alili sangapange organise chinthu mopanda kutsatira ndondomeko yake choti mudziwe police yathu imagwiritsidwa ntchito ndi anthu andale

  3. Achimwene to be a lawyer means not you know it all even the president himself is a professor of law but it does not mean he knows all zinakakhala choncho sibwenzi milandu anthu akuluza ok.

Comments are closed.