Chambo Fisheries

By October 18, 2016

Like other people wishing to celebrate motherly love, they made it to Lake Malawi not knowing they are to go back in coffins after drowning in Salima district on Sunday afternoon.

Salima police has confirmed that four people drowned in the district as they were celebrating mother’s day.

DrownSpokesperson for the police in the district Gift Chitowe disclosed that among the four, three are men and one a woman. The four travelled from Lilongwe to the lakeshore side to seek fun.

“It was yesterday when we received reports that some four people were missing and we mobilized locals to search for them but we didn’t get them,” said Chitowe.

He added that the bodies were later found floating near Boaboa cottage in Sengabay.

The police have since sent the bodies to Salima district hospital for postmortem.

In another accident, six people have died after a minibus they were traveling in overturned due to a burst tyre along Lilongwe-Salima road on Sunday.

Confirming on the local press, Dowa police spokesperson Richard Kaponda said three people died at Katengeza village where the accident occurred while three others died upon arriving at the hospital.

Kaponda added that the driver lost control of the minibus registration number NN7257 due to a burst tyre when they were traveling from Mother’s Day celebrations.
117 Comments

 1. Amatero awa ndi ausilu chaka chathanso adapanganso zomwezo . Amakhala ngati amawo ndi ng’ona kapena mvuwu

 2. Kumapita ku nyanja mutaledzela mapeto ake ndi zimenezi

 3. Zikufanana when i was at school tikalephela kumasulira mawu molondora timathethedwa as a result kumakhala kulephela

 4. Peter Cyee says:

  Mother’s something evil and it mothers donating blood to the devil, so now are u wondering about this? Each and every year women loose lives on this day yet we cant learn . Stop going kunyanja on this day dont u know that satana amakhala kunyanja? May their souls rest in peace

 5. people bear in mind it was not lake day, it was mothers day.

 6. Sad to hear,I believe not all were drunk,there is nothing wrong in going to the lake to cerebrate but rather the way we cerbrate,we must be very careful.cerebrate to praise the Lord.May the souls of our departed mothers rest in peace.

 7. Koma Malawi y? chisangalalo chilichonse sichilephela wakufa? so sad, RIP

 8. next tym try to go to church not lake things…u wont go home n coffinz..

 9. Mnyanja simukhala n’gona komaso mvuu abokho anabwera mitsinje ikadzaza especially rain season ,anthu mikiyankhura as if akufao akumva munenazo MTSRP

 10. Luwis Moyo says:

  ena azimai pa tsiku lija la mothersday anavala ma min skirt akumwa mowa paja pa salima turn off amapita ku nyanja, i think ndi amenewo

 11. Nyanja imameza sigawa kamba

 12. M’malo mopita kumudzi kwanu kukawaona azimanu koma munatengana kupita kunyanja kumakawona bonya, mvuwu, milamba ndi n’gona komanso usipa. Zimenezi ndiye amanu? Tawonanitu mwabwerako muli mubokosi amanu omwe mumakana kukawaonawo muwapasanso ntchito yolira.

 13. Mukadakhara inu mukadatani

 14. That’s what happens when you turn a mother’s day into a lake day

 15. i tink ndi chimidzi changachi ndikhalaa moyoo wautali ndithuu

 16. 1000 ways to die aliyense azafa nthawi yao inawakwanira sakanazemba in anyway so stop criticising them inunso oloko mnyumba mwanu mmomo u can die while cerebrating something lets just wish their souls to rest in peace. Amen.

 17. Kodi mother’s day ndimeneyi? Zoziyamba dala

 18. akapeleka samalandaso ndipo akalanda sama tengeso. tsikulawo lidakwana R.I.P

 19. Chisangalalo cha tsiku limodzi kudzetsa mavuto mwafa tsiku la bwino tidzikumbukirani happy mothers day

 20. Zoziwonela kukulu the results is death

 21. some people tho,ngt ndimaopa ine pano mphongo kukasamba ku nsinje nde mukati inu azimayi mpaka kutengana kukasamba ku nyanja ,matama ache amtundu chani amalawi,nthawi yolima ngt ino likhale mphunzilo kwa a zimayi ena,R.I.P

 22. Joe Banda says:

  Chonsecho Mayi anuwo munangowapatsa kachitenje Ka K2000 basi, inu ulendo kunyanja ndi zibwenzi. Shame on u

 23. Zisangalaro zasatana

 24. Thats why during moments like these i choose to stay home dziko lapansi limadana ndikusangalala too much.Rest well bangani.

 25. Ogoooo koma tsanu utengeka kwinaku dala mzosakha bwino waaa. Tsanu penyani onthuwa osiya mawanja yawo yaludandaura chosecho mwinaso wena odachita uchoka chothawa pakhomo pawo.

 26. Tsiku lana ku bala inu mumanyamuka kupita kunyanja ngati amanu ndi #mvuu kapena #ng.ona bwanji munthu ngati umawa nyadila amako sunga pite kunyanja uta ledzela ndikumaka samba nanga chonchi amayi tsiku lawo ndiku malila mudzi uzana zanzelu patsikuli amayi ama embekezela kuti mwagulila chitenje osati kwaliza tsiku lawo lika dzabwelaso chaka chamawa adzidzakumbulila inu shaaa anyway muutse muntendele madolo

 27. Hello friends, my name is Esther Mashabai was one of those millions of people living with HIV/AIDS, i received my breakthrough with the help of Doctor Abumen whom i met through the testimony of someone he has helped, after some series of conversation with the person sharing the testimony i decided to contact Doctor Abumen which i did, after some negotiation he sent me the medicine with an instruction on how to use it, i notice some change in my body when using the medicine, after completing the dose as instruct i went for test only to be confirm negative by the doctor after the result came out, words on the internet can not express it all, if you are in the same condition and you are looking for a way out of it you can contact DR ABUMEN on his email address,(doctorabumen@gmail.com), or you can call or whatsapp via +2347085071418

 28. Ndipo tizipitabe Kunyanja yimeneyo ndi nthawi yawo yinakwana dnt talk too much tmrw it will be ur ccta kukamila

 29. its a pity an advice from common peole can be taken lightly.I posted an article on my wall where i was warning mothers on this day.It is regretable as some peole took it lightly.We didnt want mothers to die during this period anyway R I P

 30. alangika ndi zintchito zawo basi guyz but R.I.P only GOD jadges

 31. Amalawi simuzatheka ndichani izi abale,, may their soul rest in peace

 32. Ndipo kwabasi shAa

 33. Chisangalalo-chinasanduka-chisoni

 34. Oukonda moyo wake ausamalira mau amatelo

 35. Most women misbehave on this day even some marriage’s were shaken on this day, I can’t believe seeing women in only t_shirt without pants, body worst full of mikanda which is not even accepted by our culture, smoking under the influence of neba, please even azunga have swimming materials of which putting it on can be safe for photos and others, ZILUBWERA mochedwa, ur were not our mothers on this day some of you but prostitute day,May God guide you and show u how mother maria was holy like. Vuto azungu tidawathamangisa msanga!!!!

 36. Vuto ndilakuti kukumapita mahule ndi anthu omwe anapeza ana apatchire ndikumadzitchura okha kuti ndi anakubala. chilungamo kuwawa koma ndanenabe

 37. Too much of everything is poisonous even honey can kill you so are your mothers happy or sad zamanyazi

 38. Hahahahaha iya nanga Mother’s day imakhala m’madzi ? Anamuuza ndani ?

 39. God punished unnecessary people
  You can’t go to the beach if you don’t know how they swim
  Only your family they will cry for you .
  Next other people you must learn from this damn mistake

 40. There were drunker and village life let them rest in peace

 41. may their mothers were floating

 42. Kkkkkkkkkkkkk chisangalalo chitafika pachimake

 43. Thank God I went to the lake enjoyed myself and come back alive

 44. pofela salambuladi

 45. anachita bwino kumila amayi ake akudya deya kumudzi .zikomo ambuye.

 46. CHIFUKWA CHANI MUMANYOZA AMUNTHALIKA ? NDINANENA KUTI OFA MAWA SADZIWIKA, OK

 47. Sad why should people go to the lake knowing they are drunk instead of spending the day with their mothers or taking them for lunch,see where this ended them.My condolences to their families.only God will judge

 48. Misunderstanding of this celebration, without going to the lake it will be somethng else different to the name of that celebration, thats what u think, and 90 percent who found and celebrate with u to that lake are not your motherz rather your loverz, other people’s wife, your girl frnd’s mother etc while your mother aliphee ku kudzula denje kumudzi kwanu uko and she doesn’t even knw about that day. If u want to celebrate that u have to celebrate in style with your mum, go to the village and celebrate with her there, kungowayendela kumudzi ko Amayi wo amasangalala akakuona kuti wawakumbukila kumudzi ko popita kukawaona!

 49. Big up man! Jst kp t up!

 50. Amakakhubuza m’madzi nasatha kusambira Chifukwa chani ? Iya zache izo !

 51. Zofuna iya nanga tiname !

 52. Ndi za azungu izii, plz asiyeni anuwake is their culture,Kumangotengeka ndi zirizonse, Munthu kwanu kulibe nyanja umvekere ndikupita kunyanjaa,FWETSEKE TATOPA NDI KUKUMBA MANDA CHIFWUKWA CHA ANTHU OTENGEEKA.MIND U!!!

 53. No one can be clever or wiser with death it’s a tym we can’t control, R,N,p

 54. Timanena nthawi zonse kuti inu anzathu amene mumachokela ku ntunda uko (akantunda) tamadekhani, Nyanja ilipo, ikanalipo, sikuti Tanzania ilanda lero ayi, kumadekha mukabwela kuno, akadzakhala pafupi kuilanda tidzakudziwitsani kuti mudzabwele mudzamile ndi dzidzukulu dzomwe tsopano, RIP! osadzayambilaso

 55. Chisangalaro kusanduka chisoni PA nthawi imodzi no one can go to swim while he/she is drink beer never

 56. Is this mother’s day cerebrations or something like drowning day’s cerebration?..#dont_drink_and_drown

 57. Need clarification here.
  Is it mothers lives?

 58. Inno Ken G Namaona

 59. malawians priority upside down even happy birthday for their kids they buy a lot of beers insteady of snacks for kids

 60. maka azimayi shaaaa!munaonjeza ndizovalazanu zamkati ngati madengu onyamulira tomato eeh, RIP.

 61. kodi its 10 not 4???

 62. Who told you that mothers day means going to the lake swimming while drunk ,,,driving while drinking beer and going out with someone’s wife and husbands – leaving mothers eating khwanya enjoying in their name,,,,,shame may God think twice where your soul”s should go

 63. kt mufufuze mwina ndi azibambo ndithu…

 64. Every month in every year in the day like this somebody might die coz of this holidy!!

 65. Azajaila umalowa m’madzi utaledzela!!!!

Leave a Comment