Teachers warned against beating learners

Advertisement
Sexual cleansing

The Malawi Human Rights Commission (MHRC) has warned teachers across the country against violating the rights of learners in the country’s primary schools.

This was said on Wednesday at Nsundwe Primary School where MHRC met with other authorities to strategize on some of the ways that can be put in place to combat physical abuse of learners in primary school in the country.

Girls are the most affected. (Image credit: www.peacetimes.news)
Girls are the most affected.
(Image credit: www.peacetimes.news)

A recent report has shown that over 13 cases of child abuse in several primary schools have been registered and have been described as one of the factors hindering the students’ education.

One of the pupils, who asked not to be mentioned, confirmed the development that his headmaster beat him and he was admitted.

“One day I wanted to help myself in the school toilets but the toilets were not in a proper condition to use so I decided to urinate on a tree when the headmaster came he asked me to choose 15 slaps or more than 10 hits in the head, when I denied he beat me such that I was admitted at the hospital,” said the learner.

Authorities have since described the abuse as one of the violations of human rights to the student.

Meanwhile, Malawi Human Rights Commission says it is putting in place ways to deal with the issue at hand to make sure that the students are safe and learning without fear.

Advertisement

130 Comments

  1. A MHRC U Shud Know Tht A Teacher Shud Use Each And Every Posible Measure To Control Th Class To Achieve Maximum Learning!Even Countries Like USA Thy Hv Not Agreed, To These Conventions On Th Rights Of Children.A MHRC, Be Teachers First, Then U R Going To Appriciate!

  2. Aphunzitsi musiye kukwapula ana mumaonjeza ngat ana menewo ndi anu ine zimandiwa muzingoyembekeza mwezi ukatha boma likulipiren ,tikulanga mwana wamweni yay

  3. Analakwa chani???? Mwanayo,,, and ana alero mukuwadziwa alibe khalidwe…..aphunzitsiwo anali amuna amamenya mwanayo?omenyedwayo anali wamkazi???….ndione poyambira uzeni

  4. tiye nazoni za maufulu zanuzo ana akuonongeka chonchi! amene uli mphunzitsi mzanga iwe uzingotuluka mkalasimo basi! mwapempha ndalama kwa azungu anuwo kuti mulimbane ndi mphunzitsi ati! #nuisance

  5. Alipo mphuzts akumenyabe ana axool? Ng@ akutopetsan anawo bwanj kungotuluka kumakagugula paja? Aphuzts gulan mafon android pliz snthaw ino busy kukhala mkalas kumaphuztsa, salary yake it? Ufulu udawachulukira anawa, mukalowa ulere2, zochta mzambr, isaaa…

  6. Inu Amaufulu Maujeni Anu. Mchifukwa Chiyani Aliyese Akakhutitsa Kosewerela Amakhala Aphunzitsi? Chilango Chilingakhale M’baibulo, Inuyo Muzingodya Ndalamazo Mkumatupa Mimba Ngat Oyembekezera.

  7. Tikusiyilani mudzawaphunzitsa ndinu anawo tiwone ngati simudzalira nawo… Munthu wakuda amanvera chikwapu ndipo ine sindingasiye… Ngakhale mwana wanga yemwe ndimamukwapula nanga bwanji enawo

  8. Wanena zimenezi ndi wopusa. Akanakhala kuti iyeyo sanamenyedwepo ndi mphunzisi sakanakhala pomwe alipa. Ngakhale Bible limanena za thyole kwa mwana wosamvera. Atipepese mwa nsanga tisanayambe sit-in.

  9. zitsilu za anthu inu a human rights mesa kuti mufike pamenepo mai anu amakupilikitsani ndi tsatsa kuti mupite ku xul mix aphunzitsinso were doin e same so dat mukhale omvela mkalasi ? thz human rights r the other contributg factors of low education standards,ngati muli ndi mphamvu osalimbana ndi a Escom,waterboards Kapena Akumatibela Misonkho Yathu Aja Bwa ? Mphunzitsi Boma Limufinye Inunso ? BEAUTIFUL FOOLS from useless organisation.

  10. Anthu awa pena pake amadabwitsa ife tikafuna kuthandizidwa samalakhula for example kukweza kwa salary malo motithandiza amangoyang’ana aaaaaaaaaaaaaaaaaa kumalawi kunali kale bola Kamuzu ndi Chilembwe atadzukanso osati izi….!!!

  11. Anthu awa pena pake amadabwitsa ife tikafuna kuthandizidwa samalakhula for example kukweza kwa salary malo motithandiza amangoyang’ana aaaaaaaaaaaaaaaaaa kumalawi kunali kale bola Kamuzu ndi Chilembwe atadzukanso osati izi….!!!

  12. Anthu awa pena pake amadabwitsa ife tikafuna kuthandizidwa samalakhula for example kukweza kwa salary malo motithandiza amangoyang’ana aaaaaaaaaaaaaaaaaa kumalawi kunali kale bola Kamuzu ndi Chilembwe atadzukanso osati izi….!!!

  13. a MHRC mungoziwa kuuza anthu za maufulu awo basi mesa ufulu umakhala ndi udindo wake inu ndomwe mwaena mukubzala mwano mwaophunzirawa mukatero muzit maphunziro akulowa pansi mukupangisa ndinuyo ndimaufulu anu osalongosokawo

  14. Ife ankatikhoma zala. Kutigoneka pa desk nkukwapula.kukadula mabanngo100. Kutola zibalo zamalaina kuzazisa dengu.kusapita ku break chifukwa cholephera masamu.

    Tidakula tidaphunzila pano ana tikualipilila fees wa mukuti ali ndi ufulu.sakulangidwa. akugobwerako ndimimba, or tikummakawapeza ku cell ataphwanya xool.

    Ok

  15. Aphuzisitu akuoneka pompa ,kulanga mwana sikolesedwa ngakhale ine ndakwapulidwapo
    Koma zina zimangoonjedza moti aphuzisi enaso amadabwa kuti mzathuyi bwanji.

  16. Aphunzotsi enaso tamva kuti akumachitisa ulesi ana kuti asiye kuphunzira computer lessons maka mmacdss chonde sinthani maganozo achabe.
    Kwanu kunatha asiyeni ana aphunzire kpmputa ndi nthawi yawo

  17. Ufulu Nthawi Zina Umaonongetsa Zinthu,mapiri Athu Mitengo Inatha Chifukwa Cha Ufulu Maphunzilo Alowa Pansi Cz Of Ufulu Wamwana Wamwano,alimbekiseni Zaufuluwawo Patsogolo Azizaba Xul Atailephera!!

  18. kulepher zanu mwayamba kulimban ndi mphunzits inu achamba eti, bwanji osalimban ndi a escom, water board ndi mbava za cash gate ngat mulib zochita ingokhalan

  19. come and teach ur children.mumazitenga ngati ndinuochenjela kupotsa teacher,ana anu zikhala mbuli zambuli.ana anu akamapanga matama ife tikhala pheee! doing our busnsses tione kt avutika ndani

  20. mkakhuta mgaiwa muzikangotaya ku thoyaz osat kubwenzera maphunziro kumbuyo.ufulu ufulu wakunyumba kwanu.iwe ndikunena iwe bwera uzaphunzitse tizaone kut suzakomoka ndizocita zaana

  21. i am Mr jang from zambia, iam really happy
    that i and my wife are cured of HIV with the
    herbal medicine of dr sule , i have
    been suffering from this disease for the
    past 3 years without solution until i came
    across the email of this doctors who have
    cure so many people with his herbal
    medicine, i also chose to give him a chance
    to help me and my wife, he told me what to
    do and i kindly did it, and he gave us his
    herbal medicine and direct me on how to
    use, i also follows his direction for use and
    he ask us to go for a check up after 2
    months and which i did, to my greatest
    surprise our result came out as negative,
    we are really happy that there is someone
    like this DR who is ready to help anytime
    any day.to all the readers and viewers that
    is doubting this testimony stop doubting it
    and contact this Dr and see if he will not
    actually help you. i am not a stupid man
    that i will come out to the public and start
    saying what someone have not done for
    me. he is really a great man contact him
    now.dr thruough whatsaap +23462447651

  22. mwana akamasokoneza mkalasi,chonde aphuzitsi ingotulukani mkalasimo,,inu zanu zidayera kale,,muzingodikira salary basi,,,mwana asakupezetseni mavuto zake izo…

  23. ife tikamawakwapula anawa timafuna kut akule ndikhalidwe komanso mwambo ndiye poti mwatichenjeza, tasiya koma m’malo mwake tizingopereka masasipeshoni kwamwana wina aliyense amene sasatira malamulo apasukulu.

  24. Samudziwa mwana awa. Ndinawamva atabwera kwa2 avekere mwana akatukana mphzts chibalo ikhale samu yovuta powereka. Chamba et! Idyani ndalamazo osathupsanazo mphunyts. Mapeto ake mufuna anawo asaphuzire mitu ngat mphondazoo iya!

  25. Simaufulu onse omwe ali othandiza.Pali maufulu ena monga kukwatirana amuna kapena akazi okhaokha,kusamenya wakuba mukamugwira,kuyenda mbulanda poyera,mwana kusaumirizidwa kugwira ntchito panyumba pa makolo ake ndi ena opitirira khumi.Sizikusiyana ndi ufulu ukukambidwa apawu.Maufulu enawa ndi oononga zinthu m’malo mokonza.Mwana iripo stage ina imene njira yokhayo mphuzitsi angachite kuti anve kapena akhale ndi mwambo ndi tsatsa basi ndipo pali msinkhu wina omwe amatha kunva ndi mau okha.Nanga poti ndi lamulo titani.Ndikuganiza kuti m’malo moti asokoneze kalasi yonse kulibwino atulutsidwe panja.Mphuzitsi akanyanyala ndi kutuluka panja kusiya ana ambiri chifukwa cha m’modzi nde kulephera “class management”kumeneko.Komano funso langa ndiloti pa maufulu amenewa ufulu wa mphuzitsi naye ndi wotani?

  26. Ma planners samva kuwawa kwa ntchito koma wokachita impliment amaimva chifukwa zikunenedwapa izi ndi bodza nde kuti aphunzitsi ambiri asiyitsidwa ntchito.muyende mma xul akumidzi mudzawone misinkhu ya ana ndi mwano umene amachita.simudzayankhulanso zimenezo.ndichifukwa chake ana akumidzi akuvutika kukhoza maufulu achuluka

  27. ooh bola ife tidzilandila learner akachita mwano ndidzikhala pa discipline ndiine…kutuluka mkalasi ndikukagona…tidzaone zomwe adzachite mayeso

  28. Even the BIBLE says “a parent who spares a rod from their children is a useless parent!” Sparing a rod from children is tantamount to killing them

  29. Kulanga mwana sikulakwa ayi,koma pali aphunzitsi ena amakhala ndi mtima wankhaza chabe,akayambana mmabanja awo uko,zose zimakathela ku ana asukulu which is not good at all,jst imagine you guyz!

  30. Popeza siwe mphunzitsi, koma ukanakhalako mphunzitsi, sukanayelekeza kulankhula zoterezi. Inuo amabungwe nthawi zina mudzayeseko kuphunzitsako kalasi ya ana 180, ndikukhulupilira kuti simudzachitaso mwano umenewu.

  31. Koma ngati zili ndalama ndiye mwasochera, kaphunzitseni nokha mukaone m’mene ana amasiku ano amakulira mtima, timatukwanidwa ndi kutchulidwa mayina ndi ana okhwefulawa,kupanda chikwapu ndiye kumupheratu mwana,mukafuna kuti tiwasiye azipanga zomwe akuna tivomera bola mwezi ukatha tikulandira!

  32. MHRC have you taught your so called learners about their responsibilities?Rights go together with responsibilities remember

    1. Wausilu iwe moti ukuona kuti ndi chanzeru kumamenya ana? Mwana ngati walakwila mphuzitsi amayenela kuitanitsa makolo ake kuti akadziwe khalidwe lomwe mwana wao akuchita pa sukulupo

    2. Iweso ndiwa utsiru kodi ungaitanitse ana angati patsiku???nanga uziphunzitsa nthawi yanji?? Poti uzikhala busy ndi makolo not your learners.

    3. Chitsiludi iwe kwabasi mesa pa xool pamakhala head teacher? Ngatidi ndiwe mphuzitsi ndiye kuti sukukwanila udzayese kudzaphuzitsa kwathu ku salima udzaona polekera

    4. @ Ofatsa ndichifukwa chake mukumalephera kufika patali ndimaphunziro bcoz usamakhale kumakambilana zoti mwana tikaitanise makolo chonsecho anakupasani kuti aziziwa chimene sakuziwa, mwanayo umamuziwa chimene ungamupangire ngati mwana simply amakhala ngati mwana wako mesa ndi kusukulu?

    5. @peter tamuuze ameneyi sakudziwa kuti teacher is the manager of the classroom while the head teacher is the manager of the school kodi akuganiza kuti timangomenya ana pa nkhani iliyonse???

    1. Mr charles sitikut kumenya opanda kulakwa kapena kumenya kwa ndewu ayi koma kukwapula kolangiza mot inuyo mwakula makolo anu kapena aphunzitsi anu osakulawitsani chikwapu?????? Be honest here kukwapula ndi mbali imodz ya class management kusiyana ndikumutulutsa mwanayo

Comments are closed.