Mozambique Traditional doctor wants to end blackouts in Malawi

Advertisement
mozambique-witch-doctor

An advert on social media shows that a traditional doctor from Mozambique is selling ‘charms’ that he claims will stop incessant blackouts in Malawi.

The doctor, Rio Lodzani, has disclosed that he is in Malawi to end challenges that have come in due to persistent power shortage.

mozambique-witch-doctor
Market red is one of the problems the doctor is stopping and its blackouts.

“Timathandiza mavuto awa: mphavu ku chipinda, chuma, kuthi­matha kwa magetsi (We help on the following problems: manhood erection, wealth, electricity blackouts),” reads part of the advert.

Lodzani has also added that he has charms to ‘bring’ lost lovers and cure many other diseases that people are suffering from.

He has since urged Malawians to contact him through his mobile numbers for the problems he has challenged to have solutions for.

Lodzani’s charms comes at a time when Malawians have been forced to use torches and candles to chase darkness due to power cuts which according to Electricity Supply Corporation of Malawi (ESCOM) have become persistent because of low levels of water in Shire River.

Advertisement

220 Comments

  1. Every nonsense people do u conclude that its weed …please weed is a good plant and i thank Jah for blessing Malawi with good natural highest grades ….uyu sichamba koma amaganixa nanga si He knows kuti aMalawi u like magetsi

  2. Abale koma malawiyu ndidzikodi kapena mudzi? Nanga mpakana asing’anga nkhani ya magetsi, nanga pakuti magetsiwa azivuta akuti mchifukwa kuti madzi ndi ochepa ndiye kodi madziwo achoka kuti?

  3. kkkkkkkkkkkkk zomwezi za magetsi mpakana iwe mfiti kuzitama kuti ungathetse shame on you we better die than bowing to you. I worship GOD alone

  4. Aka, he can bewitch any Escom worker and get them to forget their switching off magesi routine, nice; good to knw

    1. Hahahhahaa tell that sucker to end the war which has been going for ages in his portolican country and then he z welcome this side

  5. Magesi akuvuta NDE osamalemba mbwelera kuti tiziononga moto. Wa foni kuwelenga zimenezo, plz MW 24 tilembeleni za serious and zaphindu

  6. Koma inu a Malawi24 mwatipezerera kwabasi mumanena zoona koma?? Sinthani muzitibweretsera nkhani zenizeni pano ndi zokomera a Malawi osati zoti anthu angoseka mkuthera pomwepo

  7. asing’ana akumozambique pamene awona kt msika wa malbino wathesedwa ayamba njira zina zowabera anthu ndalama tieni tikhale ochenjera

  8. Komatu nde tinyozeka you tell the witch that malawi is a God fearing nation ayambe wathetsa kusavana mdziko lakwawoko and kunotu vutu lathu simagetsi koma ogwira ntchito ku escom panopa tikulingalirira zongowachotsa so dont worry please heal your country first

  9. Pachibale mukamadana, anthu apadela amalowelelapo mkupha wina mwainu , otsalanu mumaloza chala uja munadana nayeyu, same as well as the Malawian pali kusamvana ndi mtsogoleli wathu, adelaso out side the country its easy kulowelelapo

  10. Ndikugwirizana Ndi Malawi24 Pogwada Pansi Kupeleka Ulemu Kwa President Wathu Peter Pamene Ali Ku Amereca Kukatitengela Zitukuko Zankhani-nkhani…DPP Woyeeeee!!! Malawi24 Woyeeeee!!!

  11. Za zii basi. Kungofuna kubera anthu ndarama. Bwanji osamapanga zimenezo kwawo ku Mozambique komweko kuli nkhondoko?

  12. Apa Mulungu watiululira kuti tisamakhulupirire a Sing’anga ndi aboza nanga nkhani ya magesi ikugwirizana bwanji ndi mankhwala, moti ena apita akawanamize

  13. KKKKKKKKKKK KOMA MWINASO KUMUWONA SILIPASI YOMWE ALIBE OSATHETSA NKHONDO YAKWAWO BWANJ AKUFUNA KUCHOTSA CHITSOTSO CHATHU PAMENE CHAKE CHILI MMASO BWANJ

  14. Kkkkkkkkkkkkkkkkkk wapeza business yotentha pa malawi aise ma customer ndiambiri akudikira mpulumusi ngati iweyo lol

  15. akayamba kugulisa mankhwalawo nafeso mutiguliseko.. kod nde tizchekera pa ma bulb kapena pa switch kapena m’mapolo amagets athuwa?? kkkkkk kma yaa! Zafkad povuta mpakana asing’anga #MW -sazatheka

Comments are closed.