
An advert on social media shows that a traditional doctor from Mozambique is selling ‘charms’ that he claims will stop incessant blackouts in Malawi.
The doctor, Rio Lodzani, has disclosed that he is in Malawi to end challenges that have come in due to persistent power shortage.

“Timathandiza mavuto awa: mphavu ku chipinda, chuma, kuthimatha kwa magetsi (We help on the following problems: manhood erection, wealth, electricity blackouts),” reads part of the advert.
Lodzani has also added that he has charms to ‘bring’ lost lovers and cure many other diseases that people are suffering from.
He has since urged Malawians to contact him through his mobile numbers for the problems he has challenged to have solutions for.
Lodzani’s charms comes at a time when Malawians have been forced to use torches and candles to chase darkness due to power cuts which according to Electricity Supply Corporation of Malawi (ESCOM) have become persistent because of low levels of water in Shire River.
Koma amalawife amationa kupusa eeeeeh? Magetsi mpaka ang anga aaaah zachamba bax…amalaw muzacenjera liti? Fotseg
Zooooooo nama
kkkkkkkkkkkkk mpaka kuthesa vuto lakuzimazima kwa magetsi asing’anga koma dziko lili ndi mbava ili
kkkkkkkk shAme evn Sangomas fill shame 4 us kkkk u really desperate, Desperate lyk hel
Zapa thako idiots
Chingambwe
Kodi ng’anga imeneyi ina phweluka cha ku nkhotakota?
Kkkk zina ukava kamba anga mwala,sing’angayo nyumba mwake usiku amaunikila chikuni.bulutu yekha akhoza kumuvela
Hahaha! African technology. Can it really work?
MOst Welcm idea
Tell him to end the civil war taking place in his country.
Ndiamene akulodza magets ameneyo
Kkkkkkk that’s today’s life koma yah
No, he’s referring to sexual blackouts in the bedroom
Kkkkkkkkkkkk am disowning myself frm being a Malawian asaaah mpaka doctor Lozani athane ndi vuto la magetsi????? Kkkk
Paja mumasowa zotiuza agalu amalawi24 inu
Wanyela nyaupe
Mayeselo ife ai
Kkkkkkkkkk crazy world we r living
Kkkkkk He Must Be Crazy Kkkkkk
Izi ndiye zinanso
Malawian apitaso komweko
Wakuba ameneyo alibenso fundo kkkkkkkkk
mumuze sing`a nga ameneyo bolo yamake magesi ndi xithumwa xikugwirixana bwanji
Every nonsense people do u conclude that its weed …please weed is a good plant and i thank Jah for blessing Malawi with good natural highest grades ….uyu sichamba koma amaganixa nanga si He knows kuti aMalawi u like magetsi
No brain
Abale koma malawiyu ndidzikodi kapena mudzi? Nanga mpakana asing’anga nkhani ya magetsi, nanga pakuti magetsiwa azivuta akuti mchifukwa kuti madzi ndi ochepa ndiye kodi madziwo achoka kuti?
Nanuso inu mzipanga post khani za serious osati mbola imene wa post apa…..zausilu eti?…
Kkkkkk eeee
umpezaso iyeyo akukhala nyumba yopandaso magetsi….kkk
Kkkkkkkkkkkkk…….. Timva zambiritu mpaka sing’anga??mmmmh,,,,Malawi walero
Kkkkkkkkkk kma matsku omaliza zizakhalapo
kkkkkkkkkkkkk zomwezi za magetsi mpakana iwe mfiti kuzitama kuti ungathetse shame on you we better die than bowing to you. I worship GOD alone
Hahaha,,,,koma ndiye talowa nchala ndi awa omwe guys….
Zalowa chibwana
Drama?
Kkkkkkkk ha ha ha ha pwiti pwiti pwiti kha kha kha kha mayooooooo tsoko tsoko tsoko kkkkkkkkkkkkkkkk
Axis of evil…othana ndi vuti lankhondo alibe?
When The Mice Is Away The Cart Will Play,
Mwafikapo Mw!!!
Aka, he can bewitch any Escom worker and get them to forget their switching off magesi routine, nice; good to knw
Nyelo Wakenso Ameneyu Osapangila Anthu Akwawo Akuthawila Kumwanzawo Bwa?
Umakwana
Kkkkkkkk
Awaso Angofuna Kutipalamulisa. Sound Ya Mifuti Yawapengesa
Koma kukhala m malawi mkulinga uli bp mwava
Apite a ESCOM akwathu akagule chthumwacho
Simple Question: Don’t We Hv Witch Doctors Here In Mw?
kkkkkkkkkk koma Sing’anga iwe waganiza bwanji
Is that all Malawi latest news?kkkkkkkkkkkkkkkkk
To hello with his charms.having blackouts its not the end of the world.
Ndiye nkhani zabwino-ka zimenezo,abwere tikufuna magetsi amankhwala chifukwa sathimathima asiyana ndi amadzi
mufusen ngat panyumba pake pali magetse witchyo koma zoona amalawi
might as well make arrangements M-jay Styles
Hahahhahaa tell that sucker to end the war which has been going for ages in his portolican country and then he z welcome this side
haha he’s just one radical being who is trying to pull us out these blackout frustrations
Hahahaha I know this is one of malawi24 false reporting
Ndiwo Masiku Omaliza Amenewo!
Amalawi Wake Up.
Malawi is not a God fearing nation that’s irony and don’t tamper God with this mess. Fear the name Jehovah
Mumuuze sing’angayo kuti kumalawi kulibe mabvuto
Timadana ndi zausilu
Kkkkkkkk magesi mpaka asing’anga magesi zoona kkkkkk sopano mankhwalawo azigwila ntchito yanji pa mamagesi
Matatizo pa Malawi, bondia bondia ,
Ndipo zafikapa ofunika sing’anga abwelese matsenga magetsi asiye kuzima, koma ndiye angapange ndalamatu.
F**
Kkkkkkkkk koma kumeneko
Saturday lapitali Bullets 1-0 Manoma
Come and heal Malawi kkk
we will never let anyone to rob money again m’boma asing’anga asatione kupusa akabwela tithana naye
we will never let anyone to rob money again m’boma asing’anga asatione kupusa akabwela tithana naye
Kkkkkkkkkk koma yaaaah mpaka afiti zimakhuzaso za magets
Kkkkkkkkkk koma yaaaah mpaka afiti zimakhuzaso za magets
Bwanji apedze mankhwala others era nkhondo kwaoko?
Atipase Kaye mankhwala olawa kwa 2months
Arrest him, kkkk my fellow country man
Osamasuta socks kumati athesa mavuto amagesi.
U told us there’s no witchcraft in the world,izi zikuchokera kuti?
Is Dc Aquestion 4 The Normal Human Being?
Hahahaha koma dziko ili
Puss
Magesi akuvuta NDE osamalemba mbwelera kuti tiziononga moto. Wa foni kuwelenga zimenezo, plz MW 24 tilembeleni za serious and zaphindu
Kkkk! Amalawi Atipezerera Kwambiri!
Cant believe it pls mpaka masinganga kkkkkk
koma tapezeka ndithu mavuto akakula olo wa misala amakuseka
Umakwana Help Us kkk
Ndilimbikise a Escom kuti amupeze sing’anga ameneyu kuti vutoli lithe. Zikuonekelatu kuti Escom nzeru zatha ndiye asachite manyazi.
Koma ndiye kutipatatu
Koma inu a Malawi24 mwatipezerera kwabasi mumanena zoona koma?? Sinthani muzitibweretsera nkhani zenizeni pano ndi zokomera a Malawi osati zoti anthu angoseka mkuthera pomwepo
eyad ndavomeleza that one responsible 4 #blackout r witches na #ESCOM guyz.Magetsi ku mayasatsa 00:30
Hahaha koma zina ukamva kamba anga mwala
Abwere azangoyasa kudera langa lokhali? K k k Mitsitsi imeneyo..ati america yatilodza
the advert did not specify kuti athetsa ku Malawi. This is not NEWS worthy
He should go sell that charm in Nigeria.
Misala ya muvuta nsing`anga ameneyo
Izi ndiye zaboooonza magesi kumene amachokera timakuziwa tonse ngati palimankhwala ndiyekuti angabwerese ndia edzikomu only
NDE tinyozedwa
Kkk km zina ukamva mmmmh tortois lyk a stone!
Kkkkk koma Nyasaland nkhani zake.
KULOLA ZINTHU NGATI ZIMENEZO NDEYE NDIYE NDIKUPANDA NZERU
Kkkkkkkkkkkkk kma nde zachambatu
Ichi ndye chamba, akuwona ngati kuno tilibe asing’anga?
ngati alindimphavu zopanga ndalama akugulitsilanjiso cham, angopanga zambili azidya mamsomwake kobasi
Ndinkuluwiko si magesi ake awa mukuziwao ai he is saying something indirectly
Kkkkkkkk kuba uku
Can he make charms to make money lol
Zachamba
Fake
mabonya2
Kkkkkkkkkk musiyeni apange matsenga akewo tione ngati magetsiwo sadzazimanso
Mnyooo zisamba zake kapinga yemweyu
Kkkkkk kma atitoradi amalawife mpaka magetsi mphini ndye azikadula madziwo kkkk
KKKKKK koma our president akuzionela
asing’ana akumozambique pamene awona kt msika wa malbino wathesedwa ayamba njira zina zowabera anthu ndalama tieni tikhale ochenjera
Panyapake ameney akutiona kupusa et
Hahahahah zosangalatsa
Let’s give him a chance as all have failed.
bwanji ,kusowa zolemba ?
Ass hole!!!
Wangochisuta ameneyo
Zaumfiti basi
kkkk mpaka muthi mmm
kkkk kondi amalawi timawoneka,kupusa,kupepera kapena kusazindikila.imeneyi ndikhani.
Abwere basi! Zafikapa tiyesera chilichonse bola zitheke basi
Abwele akumana ndi azimayi A kumalawi using’anga umuthele achisempha chizimba angati akuganinza kuti kwa anthu atulo kuno aziwaso
Kkkkkkkkk koma misala inayi yaonjeza
Chamba basi
Malawi is the home of “BREAKING NEWZ”
Kikikikikikikiki
Komatu nde tinyozeka you tell the witch that malawi is a God fearing nation ayambe wathetsa kusavana mdziko lakwawoko and kunotu vutu lathu simagetsi koma ogwira ntchito ku escom panopa tikulingalirira zongowachotsa so dont worry please heal your country first
Kkkkkkkkkkkkk
Amalawi fodya wamkulu sitizapindula nayo.
Big Musatitole Telo Amalawife,kodi Magetsiwo Akhala Amasana Kapena Usiku Okha.Ithink Ndi Escom.
Kkkkkkk
Pachibale mukamadana, anthu apadela amalowelelapo mkupha wina mwainu , otsalanu mumaloza chala uja munadana nayeyu, same as well as the Malawian pali kusamvana ndi mtsogoleli wathu, adelaso out side the country its easy kulowelelapo
Uyu ndiye fodya wa mkulu..
How
Kkkkkkkk akungofuna ndalama zitheka bwanji
Hehehehe wopusa ndiwe wokhulupilirawe . . .
Kkkkkkkk hop Escom will hire you
Kkkkkk koma umphawi si zinthu mpaka asing’anga atipatse magetsi shaaaa
Angakhale makolo anga sadamvepo kuti asing’anga athandiza pa kuthima kwa magesi za CHAMBA BASI
Ar u sure?? Lets wait an see..
ALIKUTI SING`ANGAYO MUMANGENI AKUFUNA ALUBINO AMENEYO CHANGU PITANAYENI KUPOLICE
wabwera mu nthawi yabwino ndi mavuto amagetsi tilinawowa
Wake up my malawi
hahahaha koma yaah!
kkkkkkk koma ya man wazisakadi eeeh
I hope this is not a joke??? mpaka zafika kwa asing’anga koma!
kkkk kma nkhan zake iiiii zopwetekesa mutu
hahaha maaaad
He may be making some sense although the only true answer to that will only come from God.
What’s the difference between him and most of the christian preachers out there?
Kkkkkk ndakomoka
Doctor Nyangazidana
I don’t see any connection here.fool someone
Zaziiii.athetse nkhondo yakwao pakati pa flerimo ndi lenamo
KOmatu iye sakunena Magetsi ake amenewa akunena akuchipinda kuti panthawi yoti ukufuna kugwira ntchito mphavu zako kumafooka fooka iyeyo amathandixa
Ndikugwirizana Ndi Malawi24 Pogwada Pansi Kupeleka Ulemu Kwa President Wathu Peter Pamene Ali Ku Amereca Kukatitengela Zitukuko Zankhani-nkhani…DPP Woyeeeee!!! Malawi24 Woyeeeee!!!
Hahahaha
Za zii basi. Kungofuna kubera anthu ndarama. Bwanji osamapanga zimenezo kwawo ku Mozambique komweko kuli nkhondoko?
Kkkkkk
Paja season ya chilimwe ndi chamba sizimayenda tu, Mupengadi misala simunati.
Uku nde kutiwona kupusa
Katharina Feldmann
Ha ha
Apa Mulungu watiululira kuti tisamakhulupirire a Sing’anga ndi aboza nanga nkhani ya magesi ikugwirizana bwanji ndi mankhwala, moti ena apita akawanamize
KKKKKKKKKKK KOMA MWINASO KUMUWONA SILIPASI YOMWE ALIBE OSATHETSA NKHONDO YAKWAWO BWANJ AKUFUNA KUCHOTSA CHITSOTSO CHATHU PAMENE CHAKE CHILI MMASO BWANJ
Kkkkkkkkk eish yaaa
Vuto ndi ndani a ESCOM kapena woziwa kusakaniza zisambayo?
Kkkkkkkkkk no coment
This page is a trush with useless and unprofessional writers, I wonder its origins better shut it up nosense page!
ngiya andastenda
Chamba ichi
Tremendous madness
That’s why i hate this page… You post nonsense things
Malawi24 osamangolemba ndi zausilu zomwe,mukumatiyesatu@ #datas
Msatinamize guyz yambisan ina
Kkkkkkkk wow
1st akasake khin yamixala wayambayo then adzatitulutse mu 50 shades of darkness
Mwationjeza
Kkkkk koma achimadœooo
Zachilendo ine izi
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk wapeza business yotentha pa malawi aise ma customer ndiambiri akudikira mpulumusi ngati iweyo lol
Kkkkkjkjkkkk amalawi mpakana tafika pamenepa asing’anga kuti challenger
Uyu nde akutiseka
That’s crazy.
Asamatiyese
akayamba kugulisa mankhwalawo nafeso mutiguliseko.. kod nde tizchekera pa ma bulb kapena pa switch kapena m’mapolo amagets athuwa?? kkkkkk kma yaa! Zafkad povuta mpakana asing’anga #MW -sazatheka
Kkkkkkkkkkk ,,,,, ayeeeee the flames MW ,,, I think this ng’anga angoloza onse akudya Dora BA’s,,,,
hahahahaha ndekut ndi engineer mwina
kkkkk kma nde mwat ndizchekera mutimo? hahahahahaha
Zichekeran bora musafe nd shocko…..
Kodi zikumakhala buaj?
dekha bwana muchekera ma bulb bas kkkkk
Kkkkk
koma adha
bwanj awango kkkkkkk
Akagwere ukooo. Bola akanati alindimankhwala ophera presdent oooops i min ophera nyerere mkadagula
kkkkk koma ophera chani
There’re so many ways of stealing money wake up malawi.
Zosatheka kuno ndi ku malawi basi
Amalaw 24 mwatan tiuzen zoona osat mbwereraz
abwere basi,mwina nkuonako ku sintha.kkkkk
mwasowa cholemba ndaona
Zalowa mthabwala sono
Aaaaaaaa
This z more than insanity
kkkkkkk tazinenani za phindu mwava kkk aa malawi drama group kkk
Kkkkkkkk koomaa, malawi drama group,,wandipha nkuseka
hahaha ii man ngat ndiname man
what a stupid idea? scientifically proven impossible. Demonic traits entering the country
Bwera changu
Is It True Or Its Just Ajoke?
Ndilosauka dziko lathu lamalawi
nde chibwanatu hahah
Kikikikikikikikikikiki
nde chibwanatu hahah
Malawi wabooka, kkk