Wandale wants to be tried in an international court

Vincent Wandale

The self-imposed president of republic of Thyolo and Mulanje districts Vincent Wandale has disclosed that he is to take land wrangle issue to International Criminal Court (ICC) arguing that he cannot be charged under the constitution of Malawi.

Vincent Wandale
Vincent Wandale wants to head to ICC.

Speaking in court on Monday, Wandale said Malawi government has no power to charge any person from the two districts.

Wandale was arrested last month for mobilizing locals in the two districts to share land that belongs to tea estate owners.

He, under People’s Land Organization (PLO), was reported to have grabbed land at Conforzi tea estate.

Wandale is now answering charges of conspiracy to commit misdemeanor, unauthorized use of land, and criminal trespass.

During proceedings on Monday, the owners of Conforzi also showed the court documents supporting their ownership of the estate.

Last month, Magistrate Thokozani Soko convicted 19 other PLO members to a suspended sentence and ordered them to pay K5000 each as a bond saying the group was not conversant with laws of Malawi.

Advertisement

231 Comments

 1. Ine ndikanakonda Bambo Wandale akanapita nayo nkhaniyi ku International Cricket Council (ICC) chifukwa ndikotchipa koma ku International Criminal Court ndikodula, sangakwanitse.

 2. MR PRERESDENT HIS EXLENCE DR WANDALE SOON YOU WILL GET AWORD FOR FREEDOM FIGHTER HAMONY and PEACE!!! mulanje, thyolo your president arested in malawi

 3. Mukundiuza kuti Wandale akulamulilaso Mthalika? Ndiye Peter watule pasi udindowo chifukwa wakuwusa dziko la eni. Wakapikisane muziko mwao ndi Wandale

 4. Chamba choyamba utakula kale zipatso zake ndizimenezi.. Tamukazingileni chimanga kadabwaliyu mwina nkupungukako chamba mmutu mwakemu… Kufuna kuyesa zida eti? Kkkkkkkkkk

 5. munthu akukumenyalani ufulu anthu opanda malo inu akumwela koma mukuti ndiwoukila kma mumwela guyz simuzatheka mulibe pokhala malo ndi minda ya tea ndi macdemia nuts

 6. Gift Nankhuni, Gilbert Khonyongwa mwazimva izi koma. The president of the Republic of Mulanje and Thyolo wants to be tried at the ICC as Malawian Courts have no jurisidiction over him. Maybe the starting point should be was there warrant of arrest issued by ICC. If not Malawi will be faulted for arresting the president without wardant. That would be tantamount to provocation of a sovereign state!

 7. kwa ine akuluwa siopenga koma amene mukumunena ndinu openga chifukwa mukudziwa kunyoza chosecho anthu akusowa polima ku maboma a thyolo ndi mulanje pamene minda yambiri imangokhala sakulimamo azunguwa. kodi omenyera ufulu mumafuna azikhala ndi chiani?sangapatsidwe mulandu woukila pali chiopsyezo chosonyeza kuti ndi dziko palokha? a wandale pitilizani ntchito yanu kuti ena adzachite manyazi anthu ena atathandizika chifukwa cha inu

 8. Ndakufila man iwe palibeso …onse kwao ….no pass port asowe muno …..and immigration derpertment apa nde pali chitchito heavy ….ku army ,police,check it out malawi govermnt yinalemba mzika zamayika ena mu boma

 9. President of republic of mulanje and thyolo oriheya a vincent wandale was to take the matter to icc for judgement coz he dont trust the malawian judges,and yet the lawyer of wandale is a malawi,how i wish he was presented by mzunguuuu kkkk wandale take your time.Respect pple in authority until its your turn.how could you just wake up and say your the president of republic of mulanje n thyolo.when did you conducted the election and who declered that mulanje and thyolo districts are not part of malawi.cant you see that this is a proof to others that you smoke ganja too much?any wish you all the best your excellence kkkkkk

 10. Kod A Wandale Analakwa Chani Ku boma Mukulephere Kuwapatsa Belo Pamene Mbamva Zikuluzikulu Zoba Ndalama Zankhaninkhani Mumawatulutsa Pabelo Why

 11. If this man was from the central region, he would be charged on treason! Our judicial is too biased anf incomptent and so selective indeed not to say the least of our dpp controlled police!

 12. chomwenso mungsdziwe tili ndi ufulu osuma kwina kulikonse angakhale internationally boda ndlama, chilichonse munthu musamangoti wasuta simudziwa pa mmawa mlandu yemwe uzankomere kapena kumuwawa zolinga zake simukudzidziwa ndichifukwa aliyense anapasidwa nzeru zakezake aliyense anaphunzira school yakeyake

 13. Chilembweso anayamba choncho panaliso anthu omutukwana kuti kamalawi komweka kakhale ka dziko pakokha? cause samakapatsa mpata poyerekeza ndi mayiko ena ameme geographicaly r big, koma mwa iyeyo muli nzeru limbikila man adzadyerere ndi dzidzululu dzanu inu mutafa ife ti
  takupatsani ufulu ozilamulira

 14. timangokhala ndi mantha pa chilichonse ndichifukwa timasiyira munthu mmodzi kuti atimenyere nkhondo tinazolowera spoon feeding chilembwe anatimenyera nkhondo tinali mu ukapolo nanga kupanda achina chilembwe tili ndani leronso zikupitilira mmalo moti mzathu timuchite encourage timamubwezera mbuyo chifukwa cha mantha kuti akandiona ndili pa tsogolo boma lindimanga si masiku akale ano omangoseka pakamwa we have to express our views

  1. Inu mwachitapo chani a manzy?. Action is more powerful than facebook comment, ndikudikila mumangidwe naye pamodzi tikudziweni. Best wishes when u get urself prepared 4jail.

  2. Zoona a Manzy aone zomwe zichitike ine ndi mmodzi a amene ndinamangidwa naye Wandale ku Chichiri sanapenge Wandale chomwe tupanga tikudziwa chomwe tikupanga ngti ndi treason case tiyankhanso wapenya patali ameneyu Wandale kip it up

  3. siyani za Achilembweo anangotiyika m’mabvuto,,bola akanangolisiya dziko m’manja mwa azungu…..tikanaona kusitha pano eeeish ife mavuto sazatithela

  4. chimachitika cha mzeru ndi chani nthawi ya adzungu poti makolo anu amaonedwa ngati anyani simunamve nkhani ya livistone kuti akaona wachikuda amati nyani ndipo amaombera zina zimakhala ndi kuyipa kwake poti sukulu bwenzi ili ya ana adzungu inu mukuphunzira ku jando

 15. wake up malawi!!! dont u know that u can take ure case to the international court? whatters z money if u have money u can, chifukwa cha umbuli ndi umphawi chilichonse chomwe angachite munthu tingoti wapenga sitili masiku achisamunda ano lets wake up Malawi!!!!

  1. Mwabema vyamba imwe.. Kufuna kutchuka ndizopusa zomwe… Choyamba kukufusani ku ICC KWANUKO NDICHAKUTI…. who declared that Mulanje n Thyolo is a country on its own? ‘n when?. Kkkkkkkk kazingani chimanga mudye mmwele madzi, chipungukeko chamba. Hahahahahah

 16. MUNTHU UYU AKUMENYERA UFULU ANTHU TONSE AKU THYOLO NDI MULANJE KOMA TAMUSIYA YENKHA.TIYENI TIMUTHANDIZE.NKHANI YA MALO ADALIDI AMAKOLO ANTHU ADATILANDA ATSAMUNDA LERO TIPATSENI TAKULA . IZI ZITHA KUPONDELEZEDWA KOMA NTHAWI IKUBWERA NGATI AYESU SABWERA MSANGA.

 17. ” Malawi ” the sick man of Africa. Tanzania, Mozambique and Zambia program zikuchedwera pati? It’s high time I cried 4these countries. They are very dormant. Didn’t they not read about what hapenened with Turkish Empire? Cowards in simple word.

 18. ndimamuvetsetsa ineyo wandale komakungoti pakutindiwosawuka ndichifukwachake anthu ambiri sitimapanga sapoti komafundozake ndizoveka amalawi tiyenitiwone tisamapondelezedwe mudzikolathulomwe tilibe kwathukuwiri ayi ndi malawiyekha basi

 19. Kkkkkkk, pamenepo. Ameneyo sikuti ali yekha ayi. Ali ndi anzake amene akumuchita influence. Iyeyo yekha, angamalimbe bwanji mtima chonchi? Kumaganizatu.

 20. Hello friends, my name is Rose Sammy i was one of those millions of people living with HIV/AIDS, i received my breakthrough with the help of Doctor Abumen whom i met through the testimony of someone he has helped, after some series of conversation with the person sharing the testimony i decided to contact Doctor Abumen which i did, after some negotiation he sent me the medicine with an instruction on how to use it, i notice some change in my body when using the medicine, after completing the dose as instruct i went for test only to be confirm negative by the doctor after the result came out, words on the internet can not express it all, if you are in the same condition and you are looking for a way out of it you can contact DR ABUMEN on his email address,([email protected]), or you can call or whatsapp via +2347085071418.

 21. Please take him to mental hospital first before you continue the court hearing I believe he has some mental problem kapena if he is married afunseni akazake about his day to day life style!

 22. KWA INEYO MUNTHU UYU PENA PAKE SAKULAKWA AMALAWI ANZANGA ZINAZI TIZIONA ZOONA MUNTHU WAKU TYOLO MULANJE AZIKAGAWILIDWA MALO KUMANGOCHI PAMENE WASIYA MALO KWA ANZUNG OBWELA TISINTHE KAGANIZIDWE DZIKO NDILATHU

 23. Wat Wandale Is sayng is truth coz mw has no mandate to arrest a przdnt from another country kkkk! so wich means all politicians like APM, Kaliati, Nankhumwa, Chaponda, Mulli, Lipenga r nt malawians kkk! so who is a przdnt of Malawi? coz Mutharika comes from Thyolo! Tiye Nazo Wandale

 24. kkkk kodi President ameneyu anamangidwa chifukwa chani? nanga boma la Malawi lili ndi mphamvu zomanga president wa dziko lina?

  1. becoming a moron for claiming back his ancestors land ….. i feel he must be vindicated or wat they ate doing kiping him in jail wthout bail its a way of frastrating him …thez somaliland and south sudan they emanate from same issues

 25. What this guy is saying is true, there’s no trueth en accountability on our judges, full of curroption. Kukhala osauka sikuti ulibe nzeru or ufulu. Bell akukanizidwa, why? Look at Kamulepo Kaluwa’s speeches 2 our president, iye nde samalakwa?

  1. So are you trying to say the government have bribe the judges or what? So do you think that wandale will be able to take this case to ICC and win the case?

  2. Forget about the link, bt check out the source of this issue en hw the gvmnt is treating him, thus why he got no comfidence with Malawian courts

 26. Chimenemukumuzuzila munthuyu sindikuchiona, ndipo ndikofunika kuti amasulidwe. chifukwa munthuyu akumenyela ufulu wa amalawi ovutika ndinjala komanso umphawi,chifukwa chosowa malo olima. Amalawi tieni tizinganiza mwachangu

 27. (Zakomera kuti wakhala pakhate)ndikutathauza kuti anakakhala ntumbuka bwezi atatukwanidwa saizi kukana poti ndi mlomwe aaaaaa! Chala changa ga pakamwa.Maganizo anga Malo moti anene Za federal wangodutsira kuseli. Palibe kusiyana ndi aja anayamba khaniyi.

  1. Hahahah, guys that is insult, he is not mad yet!
   But the way he want to take the case to ICC it really proves that one day he will get mad.
   Let’s wait and see at ICC or else box 2 Zomba.

  1. What serious cases. Everyone has a right to open a case at ICC if he feel that the case is politically. The fact is do u think u can get a fair trial if the judge,court president, are the one who are against u. More over the land which is exploited belong to the citizens by birth.

  1. @OMEX uli ndichinkhope2 chonyasa ngati maliro..iweo unamuonapo munthu akumvera mphuno??? Mwina iweo umamvera kumatako…

 28. EAKING NEWS ? – Bill Gates has resigned as the ‘Chairman of Microsoft’ after receiving a letter – from peter muthalika – Dear Sir 😐 – I have some questions to ask. – Namba wan_ The keyboard alphabets are not in order, when will you launch the correct version? – Namba too_There is a ‘Start’ button but no ‘Stop’ button, where is it? – Namba tree_ I have already learned Microsoft word, when will you launch Microsoft Sentence? – Namba for_There is a recycle bin but… There is no one who comes to collect the bin. – finally eh personal question: Why is your name Gates when you sell Windows?

  1. #Dikson Jnr Kuphunda #you are insane like him too. What unpatriotic people r u? Palibe za atumbuka apa. If he was right how come all his followers have left him alone? Think twice this is Malawi.

  2. please take wandale to mental hospital, ukamasuta chamba kenako nkusiya ,umapangabe zamisala ,ithink wandale adasuta chamba nthawi yaitali, tchyolo and mulanje ara in malawi

  3. Some Of U Are Lacking Intelijent Guy Like Wandale In Ur Home District, We Have Our Own Representetive In Mulanje & Thyolo Keep It Up Wandale We Are Following U Kkkkkk, Even Born Kalindo Aka Winiko Knows That There Is Vinicent Wandale Aman Of His Integrity.

 29. kkkkkkk koma ada awa kkkk ndi ena kae bwanji asaaah. But if it were the northerners doing this people would have said they are selfish, what Wandale is doing is not different from federal system.

  1. What Madalitso Mpindamalata does on social media is to change his profile picture and he or she must be a chigoba

Comments are closed.