Malawian Catholic priest rapes teen

499

Police in Ntchisi have arrested a Roman Catholic priest for raping a 16 year-old girl at a rest house in Kasungu.

The girl is reported to have been sexually abused by Father Francis Ngalande, 44, who is a priest for Mpherere Catholic church.

RapeAccording to police, the priest was paying for the girl’s school fees at a secondary school in Ntchisi.

Thus the priest arranged to meet the girl in Kasungu as he promised that he had found a new school for her.

The two arrived in Kasungu at night and the priest arranged for them to have a rest at one of the resthouses in the district.

The girl is reported to have been surprised after the priest booked one room for both and that he started massaging her before making it to his evil wish.

The victim reported the matter to her parents who took the issue to police.
Medical report confirmed the girl was raped. Meanwhile, the priest is yet to be charged for defilement.

Share.

499 Comments

 1. Let he who has never sinned before cast a stone on this man,,,,enanu ndimamaster azigololo apa only that stinakugwileni,,NDE osayankhula ngati wansembe wina aliyense khalidwe lake ndilimeneli.inu mmatchalichi kwanu kwa azibusa okwatira spamapezeka azibusa azigololo??? Its not about the celibacy vow they made,,its the priest who has a problem if at all this whole story is not just some cheap propaganda from Mr X.

 2. Amaoneka ngati odzipereka kwa Mulungu koma amakana kuti mphamvu ya kudziperekako iwasinthe makhalidwe awo oipa, anthu amenewa uwapewe-2 Timoteyo 3:5(New World Translation Bible)

 3. Kodi usembe mumaulowa chjfukwacho sowa ntchito? Mukatopa kungo sazika kumakakwatira kusiyanandikuzjyalutsa ndi mikhanjo mumavarayo kuyipisa mpingo kumeneko.

 4. its better kumangokwatira kusiyana ndikunyazitsa dzina la “PRIEST”.Udindo umenewu umapatsidwa ulemu ndipo usawonongedwe ndimunthu amene amadzikakamiza kukhala priest pamene mtima wake suli choncho,,kuli bwino kumangokhala ma pastor basi

 5. its better kumangokwatira kusiyana ndikunyazitsa dzina la “PRIEST”.Udindo umenewu umapatsidwa ulemu ndipo usawonongedwe ndimunthu amene amadzikakamiza kukhala priest pamene mtima wake suli choncho,,kuli bwino kumangokhala ma pastor basi

 6. Munthu sanagwirire koma anali pa chibwenzi ndi mwana wa school ndipo anatengera chibwenzi chake ku rest house ku mbali ya boma ndikuona ngati palibe mlandu koma ku mpingo ndi malamulo awo apo yalakwa moti mtsikanayu akufunika awonetse chikondi pokaperekera umboni owona pa court about their relationship.

 7. Aloleni anthuwa adzikwatira basi. Zosakwatirazo it’s not biblical but just a church traditional. Mukulemba anthu Ntchito ya unsembe omwe nawo amatota, mukuganiza kuti Owen Chaima yo akavuta, adzitani?

 8. This is why i joined islam….christians priest too much lies they are doing things in their own ways not what the book of God has said……i dislike theit actions.

 9. Noboday in world can act as jesus crist.jesus is jesus and priest is priest.in this case muzingokwatila osati kumatinamizapo apa coz zaonekelatu kuti mumakhala ndi ma feelings nanunso.

 10. zimamvekanso kuti ku Vatican kwenikweniko inde ku likuluko munthu wamatama odzitcha Oyela uja ili ndi mkhalidwe lake chinsalu cha mkachisi mkudzan’ gambika tsopano zonse zobisika mkuoneka

 11. Call a spade a spade not a spade a spoon , the priest is a snake coz he had taken the poverty of the child’s family as an advantage yet dats not on, he is croock make him rot in jail for other croock priests to learn

 12. AUUZENI ADZIKWATIRA OSANAMA KUTUMIKIRA MULUNGU MUKUTUMIKIRA SATANA.SALI YENKHA AMENEYO MULI WANA MMIDZIMU TATE WAO WANSEMBE.KAPENA NDI ACHULE MAINA AWO?

 13. Mipingo inayi mavuto kwabasi imalesa zakudya zomwe zili zofunikira kwa mamuna wina aliyese lero ndiizi akugwirani mukuzembera mulungu atumiki onyenga inu wakumoto bas

 14. nde malamulo akumpingo akutinji pankhaniyi? mchifukwa chake ine ndidaona kuti sindingakwanitse kukhala wa Nsembe ndidasiya za chamba zo moti pano ndidakwatira ndipo ndikumasangalala ndi banja langa. kumangonamiza anthu zachamba, uchitsiru amenyo akhale zaka 10 osalandira mgonero Galu wa munthu. anthuwatu amangotinamiza ali ndi zibwezi zambiri. ine wansembe ndani iwe. mkhululukireni apolisi pakuti samadziwa chomwe amachita akachidziwa achokako chifukwa sali oyenera ayi, ndi wamuchunu ameneyo, kunyenga kunalibe asisiteri mkungopana amenewo bwa?

 15. nowadays,the problem is that most of our priests are not there to serve God,they just do it as a way of making there ends meet.No wonder they are not conscious when it comes to commit these shocking sins that defiles the image of the church.Please entrust people who naturally have the calling to serve God.

 16. Ndawerenga nawo ..brilliant comments and stupid ones, all in all the girl is mature And resthouse being venue, from Ntchisi to Kasungu travel, all have sexual organs and feelings ”judgement outlook eeee no word .

 17. Ngati pali church laziwanda ndiye Catholic, munthu angakhale opanda kukwatira? Paul anati ndikadakonda nonse mukanakhala ngati ine osakwatira koma chifukwa cha madama khalani naye mkazi wanu mmodzi,,ndiposo anati mwamuna sakhala kopanda mkazi kapena mkazi kopanda mwamuna ,ngakhale iweyo utakhala uphunzira olo utakhala ndi PH digree koma ngati ukusatira chikatolika ndiwe mbuli mu uzimu, chifukwa mukupembeza dragon, chilombo choopsa Papa!!! 666,muzazindikira mukazamwalira ngati mukuchita mwano

  • This is abomination yes according to both secularism and biblical nature.
   But what is done is done let the law convict the matter. And remember we all sinners none is perfect, the bible emphasized about it. A sin is a sin, either small or big is called a sin. Which is why we all dwell on earth ( the city of refuge ) as prisoners ( the sinners ). We all based on awaiting for the judgement day. We all here on earth for the grace of God except nothing and we don’t have any control over the world unless accept to be a sinner.
   NGATI ALIPO WA IFE YEMWE SANACHIMWEPO TIYENI TIKAWAPONYE MIYALA ANTHU AWIRIWA !!!

 18. Am catholic bt i wont defend the priest neither am i 2 blame the girl… Watever the situation was the priest has broken his vows of celibacy and chastity and has disgraced the church…. On the other hand condemming the whole church for the actions of 1 or 2 is out ov context…. Celibacy is a choice.. The catholic church does nt force people to enter into priest hood…. Lastly my felow catholics, christians and muslims lets not defend our wrong doings or those done by our leaders by saying w r or they are humans… W are humans and w wl never change! Xo must w keep sinning becoz w r humans?? Lets accept when something is wrong and pray for those who chose to minister the word of God that they remain faithful to their vows of celibacy and chastity in the case of priests and those who are married to the vows of marriage..

 19. Am catholic bt i wont defend the priest neither am i 2 blame the girl… Watever the situation was the priest has broken his vows of celibacy and chastity and has disgraced the church…. On the other hand condemming the whole church for the actions of 1 or 2 is out ov context…. Celibacy is a choice.. The catholic church does nt force people to enter into priest hood…. Lastly my felow catholics, christians and muslims lets not defend our wrong doings or those done by our leaders by saying w r or they are humans… W are humans and w wl never change! Xo must w keep sinning becoz w r humans?? Lets accept when something is wrong and pray for those who chose to minister the word of God that they remain faithful to their vows of celibacy and chastity in the case of priests and those who are married to the vows of marriage..

  • Mr emmanuel… Cant say much on the girl… I dnt knw if sh was induced into the act by the priest coz she felt obliged to do xo due to the fees situation…. Or it oz a mutual agreement between them in the sense of an affair…. Nevertheless having sex with the priest was wrong, watever the reason was bt if it was rape as the story claims then sh was a victim of circumstance

 20. Nkhaniyi ikuoneka kuti there is no rape case,,,umboni oti munthuyu wagwirirg sukuonekapo apa ….they have just exaggerated the title ….this must be adultery not rape…the girl z 16 and above….. These guys a Nyasa mostly lacks professionalism in gathering infor…..

 21. am looking forward to that girl 2! Some jxt wanna make history on the front page of dairly news i wonder under aged girls get into the resthouse with a man without knowing wat the rat eat when we pple sleep! ??? Dnt get confuzed anyway those who wanna be confuzed hope they r the ones who castrate priests wamukomboni azadya zamukomboni momwemo!!!

 22. ITS HIGH TIME THE CATHOLIC CHURCH STOPPED PRETENDING. All the priests to marry period. Ma sisitere ndi ansembe sikukwerana kwake. Ndipo pano anatailira akumatuluka mu convent ma sisitere mkumakagonana ndi tianyamata. Osamuyesa mulungu, yambani mwaziyesera kukula kwachikhulupiriro chanu musanayambe kupanga nao zinazi. Osamangotsatira lero ndi izi mukuchititsa mpingo manyadzi.

  • what makes it to be rape its not place,but the act.do you tell me that if aman can do sexual intercourse with a 4 years old girl in aresthouse,is that not rape?

  • Be sensible a 4 yr old can’t know sex & no one can say they agreed .14 yrs girl knows it all only age don’t allow her to be married .go around Malawi 13yrs carrying their own babies

 23. Amanama Kuti Samakwatira Pomwe Anakonda Wawo Ali Wamoyo, Chodabwitsa Akamati Akuthandiza, Amathandiza Azimayi Kodi Azibambo Palibe Osauka? Amangidwe Ameneyo. Dont Decieve People That U Are Celibate Kwinaku Mukumanyenganso. Fools

 24. Osangokwatira bwanji?kunamiza anthu basi,mungakhale ngati Paulo inu?Thats why most of are dying of AIDS.to marry is not sin.Ameneyo akagebe ndi n’kha njo wake mthupi.

 25. KUKWATIRA, KAPENA KUSAKWATIRA NDI KUCHITA TCHIMO SI NTCHITO YA MPINGO, KOMA KUCHEPA CHIKHULUPILILO KWA MUNTHU, NDIKUSATSATIRA ZOFUNA ZAMULUNGU, NDIKUMENE KUMAMUCHIMWITSA MUNTHU.GUYZ RU GOD Y UR JUDGING CHURCH?DO U MEAN KT WACHIMWA NDI MPINGO OR WY? ALMITY GOD HAVE THE JUDGEMENT TO ALL WHO R SINNES.

 26. kaya msikanayo ndi mwana kaya ayi,,,,,,,,,kaya chinali chibwenzi kaya ayi…….koma funso ndi lakakuti ” kodi wansembe amayenera kugona ndi mkazi?????”………..chifukwa ambiri ma comment anu akungonena za msikanayo kuti amakatani ku rest house??? nanga wa nsembeyo ku rest house ko amakataniko??????

 27. ,,,WHY CANT THY JUST GET MARRIED,if Peter was the first pope and was married, then the priest dhud marry too,thy z no problem with sex in marriage, but the devil manipulated the church as if marriage is wrong for the priest,old testament priest did marry,Petter married

 28. Is their any law says, that priest should not marry. The priest should resign from his position or the church should give him suspection.

 29. I only think dat they are or were in love so anayenela kufunsidwa uyo mukuti ndi teenager yo kuti amafunako chani ku guest house?

  • Nde amalowelanji unsembe akudziwa kuti sangakwanitse. Mpingo umenewu umandiseketsa bwanji, kkkkkkkkkk. Kufuna kufanana ndi Yesu? Akuti kumadzitchula kuti ambuye, kkkkkkkkkkk! Blasphemy, fire burn dem!

 30. Kudabwa kukumana ndi wansembe akudya gondolosi kuti mukudya zimenezi za chani? Shaaaaa! Mapeto ake ndi amenewa anthu amatopa awa kuteroku anangosala pan’gono kugwilira mbuzi.

 31. ndimend zimakhalila amangoti phimba mmaso kumati asembe pamene akunagonana masisteri ndi amsembe osama namiza anthu chilengedwe mchovuta ,Mulungu sanga pange mwamuna ndi nkazi iye kukhala opanda mzelu inu mwati mukhale amzelu ?ndiy mzimenezitu aloleni azikwatiwa ndi ku kwatila

 32. Any person who carnally known a girl under the age of 16 shall be liable to answer the charge ( case) of defilement. Consent of the girl is immaterial. This idiot should be punished accordingly if found guilty in the court of law.

 33. Munthu wa milungu kuusumana kkkkkkkkk mulungumwana amati chigololo sitchimo, mulungu nzimu chigololo ndichilakolako Mulungu madala chigololo nditchimo yonse itatu imagwilizana kkkkkkk apa wansembe potengela malamulo amilunguyi yadya pomwe ayimangilila koma patengela ndi Mulungu madala nde shaaaaaa mayooooooo

 34. Ansembe sakwatira koma amapanga zibwenzi, Vutonso lina ndilakuti ansembewa samadziteteza popeza they are public figures siangathe kugula ma condom kuopa owatsatira angawadabwe mchitidwe umenewu ansembe ambiri atenga matenda a AIDS ambiri akumwamankhwara ena taika ambiri ukawafunsa kuti matenda opatsirana pogonana munthu wa mulungu watenga bwanji amanena kuti polandilitsa ukalisitiya akhilisitu amatenda amatha kuwalumazala ndikuwapatsira matenda.chofunika mpingo uvomeleze ndikulora ansembe kuti aphunzitsidwe njira zodzitetezera kumchitidwewu.

 35. siyese oti ambuye ambuye kuti akalowe kumwamba koma yekhayo okhulupirika pa maso pa mulungu.monga mwana yesu kristu. Mwana bambo onse ndi ochimwa.

 36. Ku rest house amagwililira? Ngat mkaziyo amaona kti ndi mwana chomwe amakakumanilirana ku room ndi chan amaleka kukakumana ku kachisi, wamsembe unayitha coz there s n free money to a gal!

 37. Amene akudziwa kuti sadachimwepo ayambe kumugenda munthuyu…..Tikumulodza zala wansembeyu bcoz tchimo lake laonekera but zambiri zikuchitka mwanseri mmipingomu,even anthu amene tacommenta apapafe kumulodza zala wansembeyu,mukhale phee mukumbukire machimo omwe mumawachita nseri atati anthu aziwa or mwagwida zingathe bwanji??? don’t forget we are all humans..even the Bible said” do not judge” think like humans tikafuna kucommeta zinthu…that’s my vew .

 38. mm mh knena zona palpose pal zamulungu satanaso ama2mzapo asogoleli ake,evn pastas alipo amulungu n asatana,prophet alpo amulungu n asatana,cimozmoz ansembe devo alnao ake amaoneka ngat asembe kma sali comweco,nde iz mmm mh no coment

 39. KKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKK……..A Pastor mpaka kuvulira kamwana nkukapanilira ,,,iiiiiiii anyongedwe ameneyo ..mwinanso ikhare ‘ Life in prison”……

 40. Upon Judging, God Will Not Give Judgement Depending On Wheather One Was A Preast Or Not! Fonication Is Fonication So Be Warned, All Of Us Have Sinned In One Way Or The Other, Who Are U To Sit On The Throne Of Judgement.Let God Be God (judge)

  • YOU ARE RIGHT 100% but if it were ur c* child or who so eva rlated 2 u wud U just sit n watch waiting 4 the judgement dy & yet ur relative haz been abused?…..who doesn’t knw th@ thus a sin and yet u r waiting 4some 1 to tell th@ its a sin….(God gave us HIS commandments so th@ sometimes we shud knw our selves if we have commited a sin if we do not abid by HIS laws)thus adultory and if u may consult the BIBLE u will find out kut GOD’S Comandments states that we shouldn’t engag INTO ADULTORY

  • Gues Ur Right! Laws Were Made So That Whoever Bleaks It Should Face The Consepuence. This Preast Has Blocken The Law Both God’s And Judicial. Am Sure He Is Arested And Will Face The Trial, He Deserves It. What I Detest Is Lifting Heads High Commenting Obsin Language Like Others Are Doing! Let Me Say, Let God Be The Judge And The Police Do Their Work.

  • Jesus said,Matthew.23:13 Woe to you scribes and Pharisees,hypocrites!because you shut the kingdom of heaven against men,for you neither enter yourselves,nor allow those who would enter to go in.The leaders will receive many blows.dont deceive yourself.

 41. This so called men of God alwez lie to pple tht they are not allowed to marry yet plenty galfriends fo them.God gonna punish u men of God,if u knw dat u cnt make it,dnt join priesthood jst marry.

 42. Who r u fooling @catholic priests.Marriage is from God and u lie that u will serve God(if not a god)without a wife.Kani mumatotanso ?mbuzi za anthu,maula maula baxi ,bulshit mxiuuuh

 43. Koma nkhani kofunika kufufuza bho cifukwa uhule nde walowa padziko lapansi pano tima teenager to nditimene tikugona ndi akuluakulu na ngati osatipa zokwanila tikumapanga maplan ngati amenewa.

 44. This is no rape if you only knew the type of today’s girls. I’m sure the priest has been fucking this girl before someone noticed them and reported. Atsikana m’dede too much komanso akuchikonda chigololo ndiye chotilephera kuwakwata ndi chani?

 45. Vomelezani, nanuso ndinu wanthu, nthawi zina zimakuvutani, kwatilani zikatelo katundu uja ali ku thupi, siuyu tele mwakagwa mmavuto coz u wanted to cheat God, useless, tamakwatilani iya,,, ndiye bwezi ife tili nao awili awili (mitala) mxiewww

 46. Wowwwwww Kugwiriridwa Ku Rst Houz?? Iye Amakataniko?? Zimenezo Ndizogwirizana Coz Prstyo Ali Ndioffice Komwe Akanatha Kukakambiranako,iyeso Amamufuna Prstyo..

 47. Chidya makanda samalakwa kma olakwa ndi anawa cfkwa amafuna atawagulila tchipisi, kanyenya, zima- salads kmanso yogi yogi kuti adzimwela pompo osaiwala chimtuwisa

 48. That’s y apostle Paul the 1 they try to emulate said that”mkadakonda nonse mukadakhala ngati ine”meaning unmarried and abstain,and he said that chifukwa cha dama lanu kwatirani,mean if u can’t be unmarried and abstain u shud get married not being adulterous. Anthu awa ayambe kukwatira basi nyere zanyanya kkkkkkkk

 49. Praise to my God Jehovah, for making this hiden behvia of these socalled prests known. The one who is from this world belongs to it,and do worldly things. Stop comparing your selves with Jesus the mesiah, He was not from this world and He was doing things of where He was From. You! Yes you prests stop this please.

 50. Chopereka cha week ino ndichotulutsira mkulu wampingo kundende.
  Chenjezo kwanonse amene mumakonda kupereka ma k10 week ino zimenezo zisakhaleko. Tikufuna kuyambila k100 kumapita mtsogolo aliyense wampingo wakatolika Mmalawi muno. Chawona mzako chapita mawa chili kwaiwe.

 51. I hear so many protestants acting as if u know too much of course he was caught but it’s not the church which has done that u must know that God will judge everyone separately and no matter what we are proud catholics the communion of the saiths and forgiveness of sins

  • Peter,may you read John 17v11~12,people of are.kept in God`NAME not Catholic if you need salvation,that’s why He said where two or there will gather in His Name God will be available not kept in Catholic and call God`NAME it can.be Isaiah 4v1

  • There’s nothing u can tell me about the gospel u know nothing go and read history first and one thing u should know God can not lie and can not be lied we love catholic church the church of apostles and all the saints so u can keep your advice to yourself

  • My bro Peter;do you want to tell me that the church that started at the day of pentecost in Acts chapter 2 was a Catholic?The truth of the Bible cannot be compared with peoples history

  • Keep on lying yourself maybe I should agree that ignorance it’s the same as being dead if u had read history then u should be in a position to know that even st Paul himself was a Catholic so I wonder who are u to deny the truth

  • Peter, Paul was never a catholic… U catholics still offer sacrifices to priests, while Paul said in Hebrew 5 v 1-6, that Jesus is our High priest….. We dont need sacrifices anymore, Jesus did it once and for all

  • Iwe chifundo mpokoso ngati wina walakwisa mu mpingo ndiye usanyoze onse mu mpingomo ngati supemphela catholic khala chete ndipo chimene ungaziwe olo ukupemphela mpingo wina sikusonyeza kuti ukapulumuka ai nkhaniyi isiyeni akaweluza yekha mwini wake namalenga komanso mipingo inayi anthu akugwidwa ndi ufiti ngakhalenso zigololo zomwezi.

  • Iwe chifundo mpokoso ngati wina walakwisa mu mpingo ndiye usanyoze onse mu mpingomo ngati supemphela catholic khala chete ndipo chimene ungaziwe olo ukupemphela mpingo wina sikusonyeza kuti ukapulumuka ai nkhaniyi isiyeni akaweluza yekha mwini wake namalenga komanso mipingo inayi anthu akugwidwa ndi ufiti ngakhalenso zigololo zomwezi.

  • Ngati pali church laziwanda ndiye Catholic, munthu angakhale opanda kukwatira? Paul anati ndikadakonda nonse mukanakhala ngati ine osakwatira koma chifukwa cha madama khalani naye mkazi wanu mmodzi,,ndiposo anati mwamuna sakhala kopanda mkazi kapena mkazi kopanda mwamuna ,ngakhale iweyo utakhala uphunzira olo utakhala ndi PH digree koma ngati ukusatira chikatolika ndiwe mbuli mu uzimu, chifukwa mukupembeza dragon, chilombo choopsa Papa!!! 666,muzazindikira mukazamwalira ngati mukuchita mwano

  • Ndine wachi pente koma nanga azibusa akumadyesa anthu maudzu,zinjoka ndi kumapemphelera anthu ali maliseche mu dzina la yesu ndi vesi liti m’Baibulo, so apa walakwa ndi munthu osati mpingo, nanga inu mukuti mumapanga zoyenera mu ma church anu malamulo 10 onse mumakwanitsa? Tisaone kulakwa kwa nzathu kukhala kwakukulu pomwe ife tating’ono ndiye timabwaira . Mpingo sukapulumusa munthu koma ntchito zako. Konzani zanuzo pa nokha.

 52. even Pope John Paul had a secret girlfriend that woman was belong to someone so what a about priest who is he not to have a girlfriend moreover this called catholic church we already know that it’s evil thing

 53. A priest isn’t God but he cud go 4 wholes.nowadays wholes’ ranks r everywhere.by doin this he cud sin 2 God only ~not both God & government.

 54. one day God will punish them nobody cannot defeat a nutural habit stupid amukwatire huleyo osayipisa ansembe alipo ena abwino remember paul anati yemwe angathe kukhala akhale mukuzikakamiza chifukwa chofuna ndalama za mmalimana shupt

 55. Wansembeyo anagwritsa ntchito umphaw wamwanayo,mtskana anamucotsa kuntchis mpaka kukasungu ndye mwana mmat akadatan yekhayekh kudzko lakutali? Chonde pezan nthawi muwerenge pa Aroma 8:35.

  • Mnnnnnn, read the Bible very well my Freind. It’s not by compulsory to join priesthood, there are many Catholics that are married but they are serving God in one way or the other. What did apostle Paul say? Huh!!? One has to choose,,,,, and mind u God can call one to serve him through priesthood but it doesn’t mean will not be exposed to temptations. We are all human beings, what matters is how we deal with such temptations. I’m sure even your men of God be it your pastor, prophet whatever are always on a race and at battle with temptations,,,,, and some of the temptations are ourselves Christians who are meant to pray and support these but devil uses us to demolish our own Church elders. May God guide us to be good Christians that will be able to support the God’s servants. Amen

 56. are u bastard? do u think we so fool here? do u know wat does the ward rape mean? how came that bitch found in that resthouse? that’s not raping It was a mission so stop saying that!

 57. Change ur laws priesst, u shud be married rather than kumangidwa. Ofuna shud stay single bt to those who cannot manage they shud also do accordingly, its nature.

 58. Inu akatolika mumasewera ndi chilengedwe.who told u kut musamakwatire mumawononga image ya mpingo wanu,idont think kuti kusakwatira komwe ansembe ndi masisiteri amachita ndi lamulo la Mulungu ucant imagine yourself with jesus who was aprophet ov God.

  • abale mpaka lero wina osamadziwa kuti yesu sanali prophet???????? kkkkkkkkkkkkkkk mapeto ake ndizimenezitu chifukwa chakusadziwa kwanuko ndi izi wansembe waonesa mwana za mkati mwa mkanjo

  • Inu a Dan mudziwe izi munthu wina aliyese amene amamvera Mulungu amatchedwa ana a Mulungu osati kuti Mulunguyo adawabala ayi,yesu atha kutchedwa mwana wamulungu osati kuti adaberekedwa ndi mulungu ayi koma kuti adali otumidwa ndi mulungu.zikadakhala kwa mulungu kuti akhale ndi mwana akadakhala Adamu osati yesu adamu adalibe bambo kapena mayi.akatolika popemphera amati atate athu akumwamba,nawoso amadziwa kuti ndi ana amulungu.apa mwakana kuti sadali mneneri umenewo ndiye umbuli wotheratu.mneneri ndi wina aliyese yemwe adatumidwa ndi mulungu kudzalalika zaiye mulungu.pali anthu ambiri omwe mulungu adawatchula ana ake osati yesu yekha.osati poti agogo adakuwuzani kuti yesu ndi mwana wa mulungu ndi makani kakaka! Mufufuze kuti kodi umwana umenewu ndioti mulungu adabala yesu kapena zidakhala bwanji

  • Ndi zovuta kwa inu kumvetsa kuti anali prophet sinanga lero aliyese akudzipatsa u prophet thats y jesus himself said ambiri adzadza mdzina langa nadzasochetsa ambiri.mwina chizungu chikuvuta tinene muchichewa anali mneneri/mtumiki wotumidwa ndi mulungu even himself said atate wonditumayo pamenepa simunganve nokha.ibelieve in jesus than u coz u dont know as to who he was.kodi yesu samkalikira? Nanga amkalalikira zokhudza ndani mmmmmmmmm open ua eye and c

  • Whever u like it or not…JESUS, FATHER AND HOLY SPIRIT are one…thats why Jesus said when you see me u’ve seen my Father..meaning He was and is perfect 100% righteous as He’s God…by the way where did you got the imformation that Jesus is just a prophet? JOHN 3vs16 tawerengani mumvetse bwino abale mmhhh

  • #daniel though u hv quoted averse from the bible but u know nothing about jesus and i challenge u.lol jesus was father at the same time son at the same time holy spirit lol darkness at noon,koma akhristu mudasochera and simudzathekaso basi.kodi president akatumiza minister kut akamuimirire kwina kwakwe zikutanthauza kuti minister ndi presidentiyo ndi ofanana mmaonekedwe? Mulungu saoneka ndi maso iwe ndie mbuli yeniyeni poti yesu naye ankapemphera ndiye amkapembedza ndani ngati adali part of God.

 59. Ku rest house kuchoka ku ntchisi district ndikutengana wa ku kasungu district ku rest house ha ha ha kkkkkkkk
  Wapeleka money yochepa kwa huleyo wasembeyo

 60. I tend to wonder why in the first place are they not allowed to marry. there is nothing wrong for men of God to marry. after all the Word of God plainly tells us in 1 Timothy 3:2: (A bishop then must be blameless, the husband of one wife, vigilant, sober, of good behaviour, given to hospitality, apt to teach;)

 61. Timadali inu asongoleli ampingo ndye tidalila ndani ngati asogoleli ndinu mkupanga zotere komanso mukuipisa mbili yampingo plus ulemu mumapasidwa uja ukalaposo ngati

 62. 1 Akorinto 7 Vs 9,werengani ndine imeneyi.mwafika poti patsa manyazi anthu a Mulungu chonchi mukuganiza kut dzina la Mulungu lingalemekezeke,munyamula bwanji mtolo pamene mukudziwa kuti simukafika nawo. zamanyazi

 63. Here in Zambia,that case qualifies to be a rape and not defilement as charged because she was not bellow the age of 16 years.So confusing story.

  • @Maduna, Malawian laws and Zambian laws are the same. Becoz they were colonized by Britain. Under 16 is minor therefor its rape. @ Michael, i think its not good to judge a church becoz of 1 member. As a matter of fact these church members come 4rm the community were we live. Why cant we blame the community as wel? We see even pentecostal churches(born again) they impregnant each other at night prayers. To me i dont blame a church but a person. Its like blaming a company which makes cars for any accident while its reckless by the driver. Lets just conderm wrong doing. If this is a church order then report them to the police to arrest them all.

 64. Arrested for raping a 16 yrs gairl at a rest house ???? Anthu anayamba kunyegana kalekale kutopakumeneku inu muziti wagwilila muziona mbalizosekaye ok

 65. They are doing it all over the world, I thinks the problem lies in their beliefs. At some point the Roman Catholic church need to edit itself and allow its priests to marry.

  • Follow the teaching of Paul the apostle. One has to make a choice. And it’s not by compulsory for one to become a priest. One has to decide. The Catholic Church also respect the matrimonial rights and it is a blessed sacrament. Marriage life is a vocation on it’s own just as priesthood, it takes a man with the help of God the Holy Spirit to listen and understand one’s vocation. The question of temptation is always there as human beings but how to overcome them matters a lot! It is against this background that we need to value who we are as Christians by abiding to our pledges with help of the power of Holy Spirit. Amen

 66. What i knw z tht priest ndiudindo he z a human being ali ndinyere komanso teenager amakatani pa resthouse?? She must be raped,,, palibe chommangira munthu apa realise that guy out frm jail palibe mlandu apa…

 67. Inu munamva kuti wasembe satota mutafusa atate anu kuti inuyo anawatani amanu kuti mubadwe shatap sizoyalusa mpingo apa eee 16years ku rest house ku booker room ndikulowa mmmmm amafuna ukalesitiya ameneyu

 68. Nkhani Apa Isakhale Yakuti Mwanayo Wapangidwa Bwanji Rape Ku Resthouse, Nkhani Apa Njakuti Wansembe Apezeka Bwanji Ndi Mtsikana Wamng’ono Nkugonana Naye Either Rape Or Agreement