Flames into world’s top 100


Flames
Flames
Flames on position 99.

The Flames of Malawi are now on position 99 from 127 in the latest FIFA rankings released by the world soccer governing body.

The Malawi National Football team failed to qualify for the 2017 African Cup of Nations in Gabon but their 1-nil victory over Swaziland last week did not go unnoticed by FIFA.

The latest movement has indicated that the Flames are one of the best movers in the standings.

On continental level, the Flames have moved up to 28th from 38th. Surprisingly, Group L leaders Zimbabwe are on position 113 despite making it to Gabon whilst Guinea and Swaziland are occupying position 61 and 100 respectively.

Argentina remains top ranked side with Belgium occupying the second position.

98 thoughts on “Flames into world’s top 100

  1. Does it matter????and after all,we have real life issues to deal with this Crap about soccer,why don’t you fight about all these power outages

  2. Koma guys tiyen pakachitika zabwino kumayamikila team inali pa # 127,pano akuti #99 mwachiziwikile tikanangopanga qualify mu africa cup of nations tikanakhala # yabwino.komanso muziwe kuti president wa fifa ndi wina osati uja amatibela uja ai.ntchito kutibela ndalama zathu.team yazimbabwe ili pa # 113 chifukwa inaluza ndi guine one not,ndiye kumaona mbali zonse chikufunika ndikulimbikitsa macoach athu ndi ma plyer omwe aztha kumaifela game,malangizo ndioti pitilizan pamene mwasiyilapa zikomo.

  3. Koma Flames popatsilana ili number 1 ndipo matha koma khaya ndi chiyani ine ndinaonera mpira wa Malawi ndi bafana koma Malawi inali bwino koma tina chinidawa 3 1

  4. Congratulations to our boys.Let’s hope they will continue doing well

  5. Aaaaatoche apaaaa! Kodi kubereka mwana wantali, kapena wamfupi ungamutae? The answer is NO. Nde ngati udatayapo mwana oteroyo kepena ukufuna, mmmmm ndizolakwika makosana anything needs time

  6. Aaaaah very very very sad indeed i thought muzitiii aichosa mu Fifa rankings really there’s nothing good about this so called National Team waste of money

  7. Za ranking ndi zomwe ziku foliza bafana bafana a malawi nawonso busy ndizimezo ndekuwina kumeneko chamba khoboooo!!

  8. ngati tikulephera kupita ku world cup meaning palibe chomwe timatha,ma coach komanxo ma oxewera mbuzi zokhazokha,zili kukamwa mweeeee akuti kunyadira pa 99

  9. Yanga ikafika pa 99.imasowetsa mtendere,coz wina ali especially osauka amakhala buzy kuimba.Ndie ngt Flames yafika pa 99 musadabwe ndie kt yaphweka

  10. Anthu mumafuna chani kodi? Ka improvement kachitika mukuti “mediocrity” whatsover. Mumafuna ikhale number chani nanga? Number 1 or 20 ngati tinapitako ku World Cup? Ndiye muziganiza kaye musananyoze a Nyasaland anzanga inu

    1. sitikunyoza amuna but we r just reminding them kuti # 99 is not an achievement yoti tisangalale nayo panopa coz some pple ryk to settle 4 less.aona ngati # 99 yakwana sitingatsikenso and thats the case with malawians

    2. Ayi titsika ndithu amuna bola tizipanga qualify ku ma tournament sinanganso kutsika ndiye kuti mwachita bwino popikisana ndi ena osati ma periodic games iyayi. Malawi have to go ku tournament like AFCON, world Cup ma tournament oti we will showcase our talent to the world. Eeetu amuna

    3. flames sizamva by Robert…dikilani posachedwapa mene tipitile kuma# omvesa chisoni…zambiri zinatikanika..ndingoyamika kwathuko kuti zotikanika zinapangisa kuti nkhondo itikanikeso moti chokhacho Malawi amandiwaza nkhondo sizinthu.

  11. hahaha i dont appreciate mediocrity kumasangalala number 99,i cant do that,i understand tatsika ndi ma steps angapo but we r suppose to do more than that.kusangala ndi # 99 it only shows that we accept the fact that we r mediocres.lets prompt them to do more coz flamesso penapake ilibe consistency

  12. 99 zaziiiiii,maiko olimbikira ali ku top 50,xindingaxekelele zopuxazi,xizinatengere kuwina kwathu koma kuluza kwa matimu okutha mpira omwe anali paxolo pathu

Comments are closed.

Discover more from Malawi 24

Subscribe now to keep reading and get access to the full archive.

Continue reading