Mafco to start life without Richard Mbulu

Advertisement
Richard Mbulu

The news that Richard Mbulu has been banned for the rest of the season has come as a bombshell to Mafco who will face Nyasa Big Bullets without the prolific striker.

The reality of losing their best player midway through the season has likely caused disappointment to Mafco’s fans.

Mbulu has been banned from all football activities organised by Football Association (FAM) and its affiliates for the rest of the season after he was found guilty of taking the leading role in assaulting Nyasa Big Bullets players which is contrary to article 24.12 of the Carlsberg Cup’ rules and regulations.

Richard Mbulu
Richard Mbulu : His absence a blow to Mafco.

This means that Mafco will start life without their hitman who has netted more than 30 goals in all competitions for Mafco fc this season when they take on Nyasa Big Bullets on Saturday at Civo stadium in their Carlsberg cup quarterfinal showdown.

Life without Mbulu for Mafco will not be easy since the striker is one of their vital players who has contributed to the club’s good run of form in the league.

Mbulu scored 11 of Mafco’s 29 goals in the just ended 2016 Tnm Super League first round.

Why Mafco needs to plan for life without Mbulu?

Make no mistake about it, Mbulu is a very special player. When motivated he is, quite simply, a phenomenal striker. 11 goals in 15 games confirms his brilliance that’s why Mafco have to make a plan to start life without him.

Despite statistics showing the importance of Mbulu and how much he helped the Salima based soldiers by creating scoring chances and scoring goals for Mafco, his absence cannot be hardly felt if the club replaces him with another natural goalscorer.

Advertisement

119 Comments

 1. Malaiya aswede basi osawamvera Chisoni. Konseko Bb inapanga plot kuti player yemwe amamuopa asakumane naye. Ndani samadziwa ndale zakumpira. Dziko lonse liri ndizitsiru zomwe zimatha kupusitsidwa.

 2. Choka naweso wasowa zokamba eti koma anakafa wina bwenzi atabwezeretsa moyo wamunthu mbuluyo monga musilikali mpaka chitsulo kumenyera mzake siufiti umenewo

 3. Bwana George Ezekiel, kodi kuluza kwa national team yathu kukugwirizana bwanji ndi kukapanga ziwawa pa Chitowe, player akatchuka chikhale chifukwa choti akhale opanda discipline? Its not good to treat players with kid gloves coz mapeto ake zimabwezera mpira mbuyo mumakanika kuwadzudzula. Let me remind u that no body and I say nobody is above the law. FAM, keep it up! Any team/player that puts the game of f/ball in disrepute must be penalized without fear or favour.

 4. Bwana George Ezekiel, kodi kuluza kwa national team yathu kukugwirizana bwanji ndi kukapanga ziwawa pa Chitowe, player akatchuka chikhale chifukwa choti akhale opanda discipline? Let me remind u that no body and say nobody above the law. FAM, keep it up! Any team/player that puts the game of f/ball in disrepute must be penalized without fear or favour.

 5. Mungot mbuli mbuli kd mbuli imenei yapanga chan cha mpila pa malawi pano ,sizomenya anzake ndi metal bar kuli kupanda mphamvu ndiye enanu mukuti fam yakondela umeneo ndi mpila ?kd mwaiwala kt bullets inawamenya 3 -0 posachedwa pomwepa ,mpilatu umafunanso nkhalidwe la bwino plz musaononge mpila ai ndi za masewelo izi ,last year anawamenya ma noma,nao aredlions anaphanso munthu ku kamuzu stadium umeneo ndi mpila ,ku balaka nako ndikuja ana ali pa umasiye chifukwa cha zomwezi and punishment yachepa tipanga appeal agalu amenewa asadzamenyenso mpila

 6. Chi Mbulu sichinachite bwino ndipo chilango ichi cachepa ndipo akuyenera kumtumiza ku Yemen akmenye nkhondo timuone ngati angakabwereko

 7. Galu kwa eni amapinda nchira ngakhale atakhala ndi mbuya wake.Awa a chingambwe fc kusafuna kuchepa apo ndi izo amafuna kukuphan matama.Kwa eni kulibe nkuwo.mukanadzichepetsa zonsezi kunalibe.mpira waku Malawi kukhulupirira juju kkkkkkk

 8. dats a wellcome development coz in football we dont use pitch as a war field,if mbulu is a real solder send him to mwaza to protect malawians 4rom renamo solders.

 9. Mbuli osati mbulu.how can he use metal to assault his friends?

 10. Kwa ine chirango chambuluchi chamuyenera kwambiri ngati timasatira mpira khaladwe ndi mpira zimayendera limodzi ngaji kuli team yosowa mwambo imodzi mwa iwo ndi mafco izi zipangitsa kt mwina mateam kmanso maplayer paokha kutengerapo phunziro team yachisirikali yakhalidwe kumalawi ndi moyale bc ngati Luice Swalez naye anaziona ataluma mzake ndie kutenga chitsulo kukhalangati akukapha njoka Fam kep it up muzibwerabwera

 11. Zoona bac buzzy kunyamula chitsuro kuchoka salima via chitowe ndicholinga chothana ndi BB ndeno pano ndi izi mabani komaso kupeleka chindapusa mateam achisilikali mtengerepo phunziro kuti lamuro liposa mphamvu

 12. You can write a million comments accusing FAM ,but, know its only FAM who could make discissions and not you ,wait for your time to be in FAM office otherwise you are wasting your time FAM is FAM not you.

 13. Player akakhala wakhalidwe lonyasa amayenera kulandila cilango bas , matimu asilikali amatamika ndie apano atengerepo ena mphunziro

 14. Chilango chimapita kwa munthu wolakwa basii alangidye ena atengerepo phuzilo wazipweteka yekha ngati amatha amakatengeranji chisuro?

 15. i am really happy that i have been cured from HIV virus through DR.willams frank. i have been suffering from this disease for the past 2 years without solution until i came across somebody testimony, testifying about this DOCTOR who have cure so many people with his herbal medicine, “I am really happy that there is someone like DR. willams who is ready to help anytime any day. To all the readers and viewers that is doubting this testimony stop doubting it and contact this DOCTOR if you really have one and see if he will not actually help you. i am not a stupid woman that i will come out to the public and start saying what someone have not done for me and i know that there are some people out there who are really suffering and hurting their family just because of these diseases.plesase contact through this Email, [email protected] OR Whatsap him via +2348143143878. he also told me that he has cure for these diseases listed below . HERPES SIMPLEX VIRUS . COPD . HEPATITIS B . GET YOUR EX BACK AND MAKE SHE/HIM LOVE YOU MORE . CANCER . COLD SORES Thank you for your time bye.

 16. Richard Mbulu kod ndiwe amene udamuvulaza Fisher Jah man ndi anzake aja et koma ngati uli iwe eeeeish ndiwe dolo ndipo umatha

  1. said apa waoneseratu kuti iweyo ndi mbuzi n anthu amene mumanyozesa chisilam ndiinu chifukwa cha ma comment anu opanda nawo mnzeru waona munthu akunena zs chislsmuyu muziyamba mwsgsniza mpira uli ndimalamulo osati nkhondo

  2. ngat ine ndili mbuzi iweyo ndi gwape okhala thengo khani imeneyi ikugeiri zana bwanji ndichipembezo iweso ndigolo golo

 17. All the best MAFCO muchita bwino osadanda ndimakunyadirani Asirikali mulibe tswete pakalakwika mumawongola nthawi yomweyo bravo MAFCO

 18. kaya ndiwabwino koma ngati adalakwitsa alangidwe basi kamuzu adatimenyera ufulu koma adamangidwa akuganiziridwa kuti ngolakwa ndiye mbulu alephere kulandira chilango? alangidwe basi

 19. mafco olo itadxawina ho cares anyway? koma zomenya ndixitsulo dats not football amuchita bwino mbuluyo ena atengelepo mpuxilo go go ma bullets

 20. Pamenepa Atsikanawa(bb) Asangalala Coz Katundu Ameneyu(MBULU)samagonanaye Tulo,akadawapanga Zopweteka Pa CIVAL.

  1. Nkhani Sikungopanga Point Game Imene Mafco Inaluza Ayi.Inu Simudaluzeko?Nkhani Ndi Game Yomwe Ikuyembekezeledwa Pa Cival! And U Know How Prof Mbulu Is.Ndi Akatundu Amenewa!!

  2. Akhale prof ndiye akuthamanga ground? zinazi muziona musanalembe ndine wa Noma koma zomwe mukulemba zosagwira mtima mpira sindeu mpake alandira chilango

 21. Ngati kutakhala kuti kunalembedwa kuti Mafco iwina palibe Chomwe chingasinthe, ndipo ndipezelepo Mwai yapa kuti ngati kuli kotheka kuti page iyi Afam amawelengapo nkhani ndikunenetsa pano kuti ndi anthu amene amapha mpila ku Malawi kuno, ndinene momveka bwino kuti zomwe zinachitika kuchitowezo Eya sizabwino koma panalibe chifukwa chowapasa chilango chachikulu choncho ma player wo, nde tikamaluza ma Game A national team nkumadandaula pamene nokha mukuononga mpila , sindimadziwa kuti mukamakambilana mumakambila zotani , mpaka season yonse munthu osamenya mpila mutakhala inu mungamve bwanji kukuuzani kuti musalowe mu Office coz mwakangana ndinzanu wa ku ntchito kwa chaka chonse? mukamazabwera mukuona ngati mugakhagwile ntchito ngati mmene mukanagwilila kale? Sibwino kumapha tsogolo lanzanu coz inuyo muli pabwino kale mtima waumfiti umenewo

  1. Sikutitu anangodzuka nkupereka chigamulo. Zili ndi malamulo zinthuzi. Kulekerera ziwawa ndi kupereka chilango chingaphe mpira ndi chani?

  2. ngati tikufuna kupanga develop mpila,ma players ayenelanso kukhala patsogolo by developing there future pakumvelanso malamulo,malamulo salola kumenyana ndi chitsulo,FIFA imelesa player kulowa mu field of player ndi mphete ya pa ukwati,akuti ndi chitsulo ckikhonza kuvulaza wina nde a mbulu anakatenga chitsulo choposa ring,amangoyenela kulandila chilango basi…

  3. Nkhondo akafuna ili ku DRC zosewera zomwezi mpaka magazi anzawo? Mbuluyo ankafuna kuoneka ngati ochenjera pamene 40anamuimbira kumufunsa iye anayankha kuti zoti anthu amenyedwa iye sakudziwapo kanthu ndipo team yake ikufika kumene ku nkhotakota around 8

  4. Players must follow rules & regulations of football. Sikut iyeyu ndioyamba kulandila chilango ngat mukukumbuka red lions idapatsidwa ban ya 8players chifukwa chaziwawa. Adakalekerera khalidwe loti ma player azimenyana bwez kuli zotani? Lamulo ligwire ntchito kusatengera kut ndiotchuka ngat alibe khalidwe apatsidwe chilango.

  5. As 4 me i dont intertain any MDF team coz their games most of the tym samasewera bwinobwino osaphwanya discipline even ma referee amawaopa, so ma player athu asamasewele akuopa, and to me i think they deserve that punishment komaso achepesa amaenela kuwa banner chikho chilichonse m’Malawi muno kut ngat ali ndi nzeru apange zikho zawo azisewera ma soldier okhaokha…

  6. Ndipo ndikanasangalala akanangoti asilikali asamatenge nawo gawo pazampira chifukwa ntchito yawo ndikuteteza dziko komanso kutiteteza ife,osati afam atapanga zimenezo tingaluzepo kanthu iyayi palibe,ndakhala ndikuwonela pa stadium mipila asilikali akakhala ndigemu eshiii kamakhala ngati mwakandeu choncho especially akamaluzanso heyyy

  7. george iwe sukuona ximene anapanga player kut xolakwika? Ufuse anthu xomwe anayipanga #Rangers_fc yaku scotland ngat umaxitsata xampila

  8. I we ndiye mbalame heavy what would you say had it those attacked with steel bars have extensive injuries? You are a silly person who could condon violence in football!

  9. Anzao amamenyedwawo nde opanda tsogoro?, ndiposo chilango chachepa, they deserve to be punished even more, kuzimva usodya kwambiri, tizawaoneseso ngati zomwe inaona lions pa kamuzu?, ngati amatha kumenya ango joiner achina masamba

  10. aaaaah inu nde ndi mbuli basi kulemba chinkhani chosecho zaziiii zopznda nzeru nkomwe jst wasted my tym kuwelenga zopanda mutu zakozo upange delete changuchangu wamva demeti

  11. Kkkkkkkkk Koma nkhaniyi munainvetsa mmene inayendera?Guru,company,dzimakhala ndimalamulo ndengati munthu waphwanya lamulo alandire chilango basi.

  12. Jeoffrey Ndikukhulupilila palibe tsiku ngakhale limodzi lomwe iwe ndiine tidaamba taonanako nde ndukuona kuti sibwino kuamba kunyozana coz nkhani ya mpila, ndikukhulupilila kuti awa ndimacheza & aliyense amapeleka ake maganizo koma musanditenge ine kukhala mbalame coz ndapeleka maganizo anga tiyeni tipange zoti aliyense azikhala ndiufulu musazionese inuyo anzeru kuposa ena Sorry ndimatha kucheza koma zonyozana mmmm sindikwanitsa ndipo nde chisankho changa tere ngati kucheza kwanu ndikwachoncho ineyo ayi!!

  13. Sindikupanga nawo tsopano ndamaliza ntchito yanga pankhaniyi, Zomwe zimaembekezeka ndizomwe. zachitika Sorry kuti mwafa kawiri, koma sindidatukwane apo nde mundimvetse ndipo sinditha kutukwana tiyeni tidzicheza bho bho

Comments are closed.