Kamlepo spits more fire: says Auditor General’s mouth has been sealed

Advertisement
Kamlepo Kalua

Member of Parliament East Kamlepo Kalua has claimed that the country’s Auditor General has been prohibited from releasing the names of seven ministers involved in cashgate.

Auditor General Stephenson Kamphasa on Wednesday claimed that that the initial 13 files of the K577 billion audit that the National Audit Office (NAO) has submitted to the Anti-Corruption Bureau (ACB) has no names of current ministers but only business persons.

However, Kamlepo questioned Kamphasa’s independence saying his body language showed he was acting under duress. The legislator suggested that the names are there but Kamphasa has been advised not released them.

Kamlepo Kalua
Kalua says Kamphasa has been gagged.

He also queried Kamphasa’s claims that people implicated by the audit report are suppliers and businessmen.

“Do u think Billions of Kwacha were stolen by ghosts? The AG further says the names in the files are for suppliers none of which are senior government officials, are you sure ordinary Malawians have got the ability to swindle billions of Kwachas without help from senior government officials?,” wrote Kalua on Facebook.

He then advised Malawians to remove their biased glasses and acknowledge that the politicians stole money from public coffers which could have been used for important projects in the country.

“The deeds are evil whether the culprits are from your tribe, party or region. Imagine what two hundred billion can do in your district, region or country. For how long are we going to tolerate this? My heart bleeds when people look at this on regional lines and according to their districts of origin. Let us move away from regionalism and start looking at Malawi as a country,” wrote Kalua.

The legislator added that the truth will come out when Malawians get the courage to say enough is enough.

Kalua is notorious for revealing abuses of public funds by politicians in President Peter Mutharika’s government. However, his revelations on the 577 billion cashgate attracted the wrath of Mutharika who told the legislator to shut up. Kalua hit back by calling on the president to resign.

Advertisement

220 Comments

 1. Amalawi mudzuke mukugona boma ili ndi mbava kuyambira paphata paka kusi amati joyce kodi akulamula ndi joyce kodi?

 2. Ngatindizotchuka mungosiya chifuka Kalepo adatchuka kale thawi aya H. kamuzu ndemukuti akufuna kutchukacha. iyeyo Ndidolo wapa Nyasalandi auze zoona makapewa Mr KK.

 3. Kamulepo, Kamulepo uzitha kuyankhulako za nzeru m’mesa umati ukuwaziwa maministerwo lero wayamba kusintha chuni ndiye misalayo

 4. At first i trusted this Kalua guy. But when the President gave him 24 hours to reveal the names he could n’t mention not even a single name of the incumbent Minister. Basi kumangopitiriza kukamba mbwerera zokha-zokha. I have just concluded that this idiot is not serious. He just want to confuse Malawians.

 5. All the top Politicians are crooks and thieves + Kamlepoyo kungoti mwina anamumana ndipo sakumugawira ndichifukwa akumangotokota. Anali kuti nthawi ya JB? Anthu amapezeka ndi ndalama live m’magalimoti, m’mapiro, m’mchire. Mesa nthawi yobwino inali imdneija kulanda ndalama zisanaonongedwe? Zachamba basi kufuna kumangotisaukisa ndi maganizo omwe basi. Ife osauka tilibe chonena umphawi watiseka pakamwa koma Mlengi wthu alinanu chochita azathanananu pomaliza

 6. These r unofficial results.The names r stil contiuneing.1 thing i know is that God is watching & wen he wil speak u wil b in hot water.Mulungu sangangotisiya chonchi ena ndikumatibera our taxes.

 7. Kape wina ali buzy kusapota kamlepo ngat ali olimba mtima osangetchula mainawo bwanj,,,atumbuka dyera,kuzikonda muzafa osaona mpando wononawo kamba ka zimenezo..zindere za wanthu ,.,…,ma folena ngati inu ngat zikukunyasani osamapita kwanu ku DRC bwanji kuda ngati manyi agalu……

 8. Keep it up Kamlepo we need people like u in Malawi, we are tired of being fooled by stupid politicians who think they are clever if to die we will die together am 100 percent behind u. Mbuzi ndi iweyo ukusekelera kuti anthu aziba ndalama za bomawe mwina umadya nawo mumangidwa limodzi.

 9. akhale dolo osangoulula bwanji?u you dont kno Kamlepo anadikilitsa anthu mu 1993 kut aulula zokambirana zoopsa zomwe Ngwazi ndi nduna zina eg a Tembo a Deleza a Bwanali ndi ma seniors ena like mai Hilder Manjankhosi koma ai sanaulule mpaka tinavota kkkkk only fools of this generation pays mo attention to his big mouth,akhale wachilungamo why sanadzudzule alamwake aja Joyce Banda bwanji kuti naonso awononga dziko?watch out this man he got a sweet talk like a snake,he speaks like he got masters degree but he dont have even a single degree he speak as if he truly hates tribalism but him is so tribalistic no1.he failed many times n now he is seeking yo attention so that he can gain more millege, why MCP is quite on this only him n Harry Mkandawire are boiling why?

 10. Kamlepo ndi chindere Chakufikapo iye popeza akuwadziwa anthuwo osawatchula bwanji? Kodi report limeneli ndi la chinsinsi kapena kuti silinatuluke? Kape uyu watikwana ukhale munthu osanena kuti tikamatche kuti Joice abwere . Ndiye zina zofoila kumavomeredza muzachenjera liti

 11. Musiyeni Ndiwamisala Uyu.Chitini Chopanda Kanthu Chimapanga Phokoso.Awafunse A Ujeni Ndi A Ujeni Adali Olongolora Kwambiri Munthawi Ya Bingu,pano Adagwa Chagada Pa Mpando Wa U Mp.Ngakhale Ndalama Zobedwazo Zitabwezedwa Palibe Chomwe Ife Amphawi Tingapindule.Iwe Kamulepo Useke Kuchimbuzi Kwakoko Ukutinunkhitsa Mkamwa

 12. Vuto anthu a Dpp umbuli akuvonerza bwapini zopusa simukuziwa kathu agalu inu anthu anaba ndalama hule kaliati,chaponda,Musa,Gondwe,Kondwani,kalirani pamozi ndi bwapini sopano mukuiwara kt anthu kt ndindalama zanu zomwe akukuberani segulani maso musamunyose Kamlepo apa

 13. A Kamlepo, kodi inu makungoziwa anthu ndimaudindo awo okha osati mayina awo?? Ngati mukuziwa maina a nduna zakubazo tangozitchulani. anzanu akuti nduna mukunenazo sakuziziwa, ndie inu ndinu amene mukumabwera poyera ndikumauuza mtundu wa Malawi kuti mukuziziwa ndunazo. What fails you to mention the names of cashgaters?? What u fear z what those dont know the names fears. Ngati inuyo mwalephera kutchula wina angawatchule bwanji poti woziwa anthuwo ndinuyo? Mukalephera kutchula ndikutengerani kukhoti

 14. Reveal o shut d hell up.Wasting hr time wt childish politics.U only de 1 purpoting 2 know tha truth.Act courageously as u speak.

 15. Only intelligent will understand Kamlepo.Only intelligent will understand Kamlepo. If it was in court, I could have said, Auditor General has convicted himself. Names of companies are in the report and no government officials were involved. If I have a company, can I pay myself twice from goverment account without delivery of service? who authorises payments?

 16. Charles mwanawa sefura Mwangolera. Mr.kamlepo.gwiranchito amdara bina Malawi tosetili namwe ndipotilitekhayayi Chiuta walinase pamoza mpakaunenetso usangikenge nabo nabo mwenabo twakataramwe ndukomwe mubomabingiraghalulu lelopofika pazovatake potosabapokwangura nduko kamlepo

 17. I salute the man for coming up loud! We need whistle blowers like this man,as brave as he is!
  Now the issue is out there, its up to Malawians to rally behind this man to unearth the truth!
  We would like all implicated parties to be brought to book!

 18. What kamlepo can see while seating some of us can not see it while we are standing on top of a highest mountain.let mr president give kamlepo an AG seat so that manyazi azamugwile ngati akunama.

 19. Sono ka ku parlıament east ndıye kutı kodı? Kwenıso nganya usange wanthu awo ukuwamanya waulure waka kası mukabıranga lumoza tax payers money nthewe ızı.Musazabweretso kwathu kutı muzatısokoneze kutı tızakuvoterenı mwalemba mumajı vyaka vake nı vıno nase tılıkujulıka kumaso nkhanga ızı.They just talkıng kak every fuckın day.Tavuka nanu fuck sek.

 20. Chilungamo chiyenela kuyenda ngati madzi,anthu nziko muno tikuvutika chakudya ndalama zikusowa komanso zinthu zingokwela mitengo kaamba ka anthu amenewa.nde munthu wina wapezeka wolimba mtima woulula anthu amenewa inu mukumulesa why?musiyeni awulule zomwe zikuchitika basi,

 21. this guy is mad one 😀 once he say he got names now after failing to release the names..he put blame on AG..aaa

 22. If the mouth is sealed yours is not then come with the list and nobody will blame you for doing good. If not then you are making unwanted useless noise

 23. nduona ngati kut position iliyonse has distinct duties. nde ngat kamlepo akufuna ena atuluse mainawo, it means that imeneyo ndntchto ya amene akutchulidwayo (auditor general) we are not supporting kamlepo, why? still sleeping? kungodikra ena atiyankhulire??? aaaa iyayii

  1. koma zodana ndkamlepo chifukwa chot akulankhula sizoona ayi, ineso ndulankhula “auditor general taika pa air onse amene akukhuzdya ndzauve zoba ndalama za anthu osaukafe”

 24. tiyenazo mr kamlepu pitiliza kuwasokosela atulusa mayinawo,”pachokopachoko kurya kwa ngata”..NOTHING 4 US WITHOUT US!!Leave Mr man asokosere mmene angafunile & let’s suport him..sangatuluse mayina ngati ife tangokhala duu aziona ngati sizikutiwawa

 25. I think Malawians have got a problem, ndale za pa mtundu. Just because DPP is a lomwe dominated party all lomwes do not see anything wrong if the dpp top brass stole our money. Corruption ku Malawi siidzatha because even poor people are supporting it just because those who stole money are from their tribe. Zamanyazi.

 26. Amalawi ife sitimva timafuna anthu ophunzira lero siizi.Akamlepo zomwe akunena sizoti achita kuuzidwa ai.Ndi zinthu zoti zili patebulo ya anthu ambiri,iwo akungochita manyazi chifukwa nduna zomwe zatchulidwazi.Atsogoleliwa saganiza zaamalwi,iwo amachita ngati amakhala kumwamba talira kokwana anthufe.

 27. How can i explain this testimony of a great man who cured me from HIV virus. i was HIV positve for 3years, until i saw somebody testimony, testifying about this great man DR.willams frank on how he cured him from this virus for 7years.them i contacted him through the Email the testifyer drop on the internet an he respond to me, an ask me some question. after that he gave me some medicine that i take for 7days, after 7days, i went for HIV test. Behold i was tested HIV negative, God bless Dr.willams frank for healing me. if you are face any problem or any of your famaily are HIV positive, please contact him through this Email. [email protected] OR whatsAp him via +2348143143878.

 28. Those who say Kamlepo should take the names to ACB are blind. ACB is not independent. Audit reports are supposed to be published. Why is the Audtor General failing to do so?

 29. I hope there is no truth what this honourable is saying if we will continue to follow him he will simply mislead us.

  1. musakaike ine ndudabwa nayeka aaaaaaa osangokhala phee bwanji ndikudikira what next than kumangoyakhulabe angotiuza intesion yake ….

 30. HE WAS THERE B4 CHIHANA,BAKILI,BING U,APM,…. MR KAMLEPO HAS NOTHING TO OFFER MALAWI GOING FORWARD,HE IS A RECYCLED POLITICIAN,HIS TYM IS PAST,HES A CONFUSIONIST,FAILURED POLITICIAN,… OMUMVERA UYU NDI A BAKHA,A TAMBALA AKUDA,MA LOKO OTSEGULIRA CASHGATE,… TO HELL WITH FUCKEN KAMLEPO,WHOSE SON IS BUSY MAKING SATANIC MIRACLE MONEY WITH BUSHI… T!!

 31. Ngat che kamlepo ali ndi mayinawo angoyamba kulengeza basi,,,palibe nkhani apaa,,palibe Wandale amene ali wabwino onsewa ndimbava basi

 32. This stupid mtumbuka he is seeking 2much attention from the media idon believe his mickey mouse party is still existing idiot toy president.mtumbuka will never be the president of this country

 33. Mbuzi ya Munthu Kamlepo,u always want peoples attention,grow unatinamiza uli ku Joni,now grow and practice matured politics or shut ur mouth.

 34. Muli mmudima bwanji mukubisa nyale?Malawian…#bitches!Quiet! Quiet!Quiet!Quiet!Quiet!Quiet!! Hey #Haters Quiet……!!!!#UselessHaters!..Quiet!!! Kamlepo akuwunikira inu nomwe amene muda udzidwa kuti mudzikapha mbewa ndi Ziwala akoporo anthu osayamika zabwino zomwe Munthu woti si mubale wako akukuchitira still mukufunafuna kumugwetsa Mphwayi!!Anthu afiti inu!

 35. Kamlepo you said you knw the name why cant you mention them your mouth has also been sealed?? Then dont blind Malawians while you have chibanzi in your mouth

  1. Do you think he is the right person to mention those names?In your own understanding do you think someone can go and steal tax payers money without the help of government officials?

  2. No you can’t steal tax payers money without the helped with or government official’s but kamlepo’s right Dango Gondwe you know the problem of the people’s no nothing about government system but only know talkertive

  3. sikumudzi kwanutu kuti umangodzuka ndikuyamba kuulura. Umaudziwa mlandu wa defamation ndi azinzake? Think again b4 u blame kamlepo.

   As much as one might be willing to go against the president and other people for good of the country, Its not good to die for this country.

 36. Kulemc kwambiri nkhani za kamplepo kwanditopesa ine owerenga.kodi iyeyu mukumuthiramo ngati ndani?munthu uyu wakhala akulephera pa zisankho kwanthawi yaitali,wangolawako ulendo uno basi nkumatikwana chonchi? Kodi sakuonanso chabwino china choti anganene? Akula bvumbwe otantha patsekera.

 37. Mr Kamlepo ndinamandwa!
  Mukudziwa kale!
  Adayamba pobadwa!
  Mukudziwa kale!
  Muli mmudima bwanji mukubisa nyele?
  Mahaters Ali useless!! Kamlepo akuchitani dzinthu!
  #GocatchgrasshoppersandRatsbitches!

 38. 100% True! Auditor General’s Mouth Has Been Sealed.
  “Amachita Kunjenjemera M’mene Ankayankhula Pa Mbc tv Bodza Lakelo.Bodza Limazunza, Pomwe Chilungamo Chimamasula”.

 39. Akungofuna kutchukirapo uyu asatinyate nalo phula mmaso ife simbuli ayi.akuyesayesa kuteteza amayi potembenuza nkhani uyu,ngati akudziwa maina osawatchula bwanji?anthu aziti Kalua ndi olimba mtima,ukunama koma malawi adawona sopano ino sinthawi ya Kamuzu ayi.uthokoze kuti APM ndi lawyer komaso wodekha akukuwelengani pamenepo.

  1. Ndiko kupeperako kumeneko,akadakhala wombwambwana akadapambana nkhani zonse ndkupambanaso chsankho ali ku chipani chotsutsa?MCP ndiliti idayamba kususa osapambanapo ngati mtsogoleri wake ali ochenjera?look into it amwene,ndiumburi womwe mukuonesawu akulu.

 40. This man just likes arguments and being in the news. If he has the names and is as brave as he claims why not just bring them out. This is going round in circles and not moving forward. Surely all Malawians will be happy to know the names. Only then can we truly tell APM to fire them otherwise we have no leg to stand on. Does APM just pick and fire ANY 7 from his cabinet? Let’s be real.

 41. Kamulepo ndi dolooooo!!! Tiyeni nazo Sibweni tipex anagwira ntchito kufufuta maina aja koma la minister ujayu lilipo lili kutseri kwa last paper so Kamphasa sanaliwone

 42. Tiwapemphe a Kamulepo Kaluwa kuti mukazakhalako President chonde muzamumange Muntharika.Ngatitu nkotherkera ngati mungazaulaweko mpando wononawo muzatero.Panopa mukukhala ngati mukusokoza kulimbikila mtunda opanda mazi.Mungoyimika chilimika kuti 2019 ngati zingazatheke muzapambanenso kampando kau MP mukazapusanso azakulandani anzanu ndiye kaya muzikasokosanso kuti kaya simuzamvekanso ayi.

 43. kampule ndi kape kwabasi mesa amupatsa mwayi oti atchule mayinawo nde bungwe lawolo2 ndilopanda phindu nde asatisokose ngati satchula ndibwino asankhe kukhala chete chimbava chachikulu ndichocho nde inachipweteka chinatuluka opanda kanthu zako zimenezo ife siandale2

 44. I fk the man is stpd wth a rotten mouth. Wy r u failng 2 relz the names urself yet u wot others to do so 4 u.

 45. m’malawi mwachuluka mbuli wat wrong kamlepo z done he refuses gov.to mention de pple who r invoved in cashgate nde ndkulakwa wow wow wow akadali kutipondelez tiyen tiyende tiphuzre zinth kamlep y gd

  1. Amos Mika, its beta 2 b a ticha than u olowesa chinamwali mmudzi.We pay tax,amalume ako ndikumaba.God is watching.

 46. Amalawi tizafa Ndi umphawi chilichoso mbasi God is watch kumuyese mulungu basi azanu aku lemele amaga ma big deni Motown kuzela mu cashgate work up Malawi .stop saying God is watch palizithu zina zowoneka Ndi maso lets handle these by supporting kamlepu

 47. I think Julius Malema is better than Kamlepo Kalua coz juju guy is brave, courageous and strong personality while Kamlepo is just consuming his time 4 nothing, just reveal if know the names of rotten Cabinet ministers

  1. malamulo sakumulola man.kod nde kut muzingoombera manja zilizonse? kod tinamuvotera ndi ambiritu koma apapa zanyanya tisawade akaluwa usi sufuka popanda moti

  2. And south Africa democracy is vry mature wea no1 is indeed above e law . cases r handled accordingly despite political affiliation

  3. But AG and these rotten ministers are sons and daughters of APM so how can AG name them? Its very hard as long as DPP is still rulling malawi for them to be revealed even Kamlepo also is just consuming his time. Panopa Andale ndiakuba

  4. Aaa kamulepo ndiofoila amangotokotela kumbali kma ndiwamantha bad,you cnt even compare with the clever 1juju bro,amene uja sioyelekeza ndimphwepwa zinazi,akanakhala kamulepo kt alindikuthekel pandale sakanat azingothuluma opanda sopprt dzaka mkumatha uku akulamba ai.Amene uja ali ngat galu ongokonda kuwuwa kma mano alib,amadyela momwemo

  5. I don’t condone any type of corruption and yes indeed those involved in this cashgate thing must be brought in the open and be probed, but the Mr. Kamlepo Kaluwa’s noise is questionable because Kamlepo is well known to make noise when he he needs CHIBANZI to feed his stomach. He used to threaten the former president Dr. Muluzi like “ndilowa m’tchire” on trivial issues. Such men can’t be trusted when they make noise. If there is evidence about the names he knows then there is no harm to reveal them. If the argument is like he is afraid of malamulo then the same malamulo will protect him or should just shut up and find other means of getting CHINTUWITSA

 48. Chilungamo sichingadziwike pakalipano, pokha-pokha uyu apereke maina ndiye uzaone kuti chilungamo chili pati. Kodi presidenti ali serious pankhaniyi kapena ai, ndiye ungadziwe chilungamo chake. Pano zivuta chifukwa nayenso gwikhwi uyu, akukanika kupereka kaya amafuna kutchuka kaya ndichiyani fisi ameneyu nayenso ndi misala yake yosanthayi.

 49. Pa Malawi pakanakhala anthu osaopa kunena chilungamo ngati kamlepo bwezi bwampini akumva juuu sibweziso usilu wakewo akupanga koma amalawi mantha akuti azafe ndi ukalamba ngati khwangwala lelo ndilimenelo dziko latsala mafupa okha…jeez anthu oipa

  1. GUYS osamango sokosela nga nkhululu Kamlepo akunena chilungamo iyeyo okunena zomwe or mwana wobadwa kumene atha kudzuwa kuti nchilungamo nde mukuti aulule, iyeyo ndi public protector? Anaba ndalama zili kwa boma la dpp kuulula kapena kutseka anthubpakamwa ndi makobidiwo, koma chosangalatsa nchakuti ndalama za anthu ubvutika ukaba ngati suzisiya nde kuti zitha ngati makatani. Asangalale lero abe misonkho yathuyo ayaembekezele kukanthidwa.

 50. Honestly this Kamlepo guy is fearless. He is not a pretender. Unfortunately he is not supported because many people are afraid ( cowards even ). I remember how in the 90s he used to speak fearlessly against the dictatorship of the time

 51. Peter muntharica ali mgulu pa list nde mukuganiza kuti angapereke mainawo???? chala sichiloza mwini apa zavutapo mungochedwa pezani zina zoti muchite apa zavuta ndithu apa

 52. I know that what kamlepo is saying is the truth…..nothing but the truth…..this name are there,

  akuwateteza mwakathawi kochepa…..though I know that they are living in fear where ever they are!!

 53. I now believe this Kamlepo guy is clever for nothing, why busy castigating others for not releasing names of cabinet ministers involved yet he claims to know them? why can’t he just mention them so that the issue should stop making headlines. otherwise we will deem him a fortune seeker while fabricating stories.

  1. this guy is not fabricating stoeies he know what he know the only thing he is lucking is confidence 4 em to be competence herolic justince fighters familly like julious mamlemya

 54. how difficult the economy of the jungle might be, but only a lion will never eat the grass, so APM won’t realese those names, it is impossible like a lion eating grass!

 55. During PP era, they failed kuchita investiget and reveal the names of the said ministers. Lero ali ku opposition komwe akhale 100 years to come then they want the names to be released. That can not happen. Wauzidwa kuti apitise mayinawo but angotokota. So what do you want. Ulibe umboni weniweni.

 56. Though am a DPP, but I think there is sense in what this man is talking. We Malawians are coward, we are not couragious enough to fight corrupt people especially if they are in govt. Why cld Kamphasa fail to clarify 3 Months ago when people started allerging the Ministers? I think we must support Kamlepo if we really hate corruption and want our money back. DPP woyeee!

 57. Kodi KAMULEPO KALUWA anabwela bwanji ku Malawi ofunika aonetse mapepala ake mwinanso anapanga expire choncho ayenela kubwelela kwaku mpoto bwenuuuuu
  – Ife a Malawi amene tili kuno ku Zambia, Mozambique, South Africa, Swaziland, Zimbabwe, Kenya and England choncho tikupepha BOMA kuti Kamulepo Kaluwa amangidwe kuti akanene zoona ku mtundu wa Malawi. AMEN

  1. amene mukumuda kamlepo nonse ndinu mbuzi munthuyo akayankhula za mtundu wa amalawi sakuti alomwe kapena achawa kapena atonga kapena ankhonde ayi pulizi sukulu simatha yesani kumphunxzila chifukwa enanu ndi mbuli zopita ku sukulu

   1. James mkoko ndiwe mbuzi eti iwe umazitenga ngati ndiwe yani iwe ndi kunja komwe suziwako ngakhale pa Mozambique pomwepo pakukukanika galu iwe who are you to say kamulepo amumange. Kaluwa akunena zoona pitala mathanyulayo akukana chani akuziwa kuti akangowamanga athuwo iyeso upresident watha ndiye osamangoyankhula ngati mwasuta chamba. Muzingokhalira yomazipenta blue mthupi mose thawi zonse kumbuyo kwa malore kupusa kumeneko.

  2. You’re just talking senseless about Kamlepo to show his papers, what papers. Let’s come to the truth of the cashgate, the president is n was trying to interfere all those who got evidence including the auditor general. We have to fight for the truth why you want to sit on it how long will we be watching our beautiful country to remain as it is. Halalaaaa Kamlepo we are all behind you and the entire world’s watching

Comments are closed.