Kamlepo gives Mutharika 24hours to resign

Advertisement
Peter Mutharika
Kamlepo Kalua
Kalua orders Mutharika to resign

Opposition People’s Party Vice President Kamlepo Kalua has given Malawi President Peter Mutharika 24 hours to step down.

In a Facebook post, the vocal politician has told Mutharika that he has 24 hours to make him the attorney general or the ACB director so he can name cabinet ministers involved in corruption. The other option for Mutharika is to step down.

Kalua has been alleging that seven ministers in Mutharika’s cabinet have been implicated in a report on Cashgate activities that spanned the reigns of Bingu wa Mutharika and Joyce Banda.

Kalua alleged that he knows the ministers and Mutharika was shielding them.

However Mutharika dared Kalua to name the ministers or shut up.

In return, he (Kalua) has said that he can only name those ministers if he is the attorney general or director of ACB. He has therefore urged Mutharika to appoint him to those positions or step down.

“The files containing these names are with ACB, Auditor General and Mutharika wants me to name? Fact remains that Billions were stolen by people some of whom are ministers today! Therefore I also give u 24hrs, make me Attorney General, make me head of ACB and I will name with the immunity that comes with these positions, if you don’t, you should resign Sir!” he posted.

More than half a trillion of public funds disappeared through cashgate.

Advertisement

674 Comments

 1. What more can i say is that i love Mr Peter mutharika coz he’s trying make malawi to have a better project of (roads) kamulepo you have to put some respek in his name…i salute Peter mutharika

 2. kamlepo is full of blood politics, doesnt know 21st century political ground…..get a rest mr. kamlepo we r tired of ur nonsense tongues…..kukoza zinthu sikuopseza ai nids calm ……contact n dialogue officially

 3. bac kungozuka ndi mbwelera zako kamulepo 24hrz yachan dont bram dpp coz iz zinayamba kale ndie ler kumalimban ndi peter u must vry shupt anthu ngat inu ndi aja mumayambisa ziwawa ndie mulekeletu kukamba za ppm ndi boma lake.mesa mukut kukubwel 2019 ndie osangodikil bwanji?????.

 4. It is true that he must resing bcz he make our country more poor, it bcome like zimbabwe now which is not goog.

 5. Vuto ndi loti people don’t knw the background of kamlepo dat he is a mad person,which mean his followers are mad as well.viva DPP viva APM

 6. Ithink kamlepo is a very stupid man, he himself said dat he knows the names of dpp ministers who are cashgaters and the state president gave him a chance to mention the names to the public and he is saying aah no! Siudindo wanga kutero nde nanga amaziyambiranji? Nanga kwenikweni chomwe akufn ndichani? Nanga akuopanji osatchula mainawo?

 7. Mudziyamba mwanganiza. Ndani kumalawi kuno angalole kutula pasi udindo? Anavutika yekha kupanga kampen who r u to step down APM.Where r u when he took over the office of president inu mungayendetse dziko?kaduka bwanji ngati mukulephera kutukula ku dera lomwe mukuimira what about dziko bonya.

 8. Kamlepo is ready to mention the name s.Apoint him as Atonny General of ACB if you jump simply means you are defending those thieves in your cabinet. Or else stepdown.yet you have done nothing for Malawians. Better your brother Bingu, but had pride.

 9. Eee komatu galu samabereka mphaka mumene akuzudzira anthu a DPP wina kuma supporter chochi anthu akumwera ndiwopengadi stupid Dpp supporter’s Including your leaders

 10. Lets be spacific ndale ndi masewera chabe anthuni, imagine nkhani ya cashgate inayamba lija ndi kale moti ena utsutsa boma pakali pano ali muzitokosi, and otsutsa ena ali pa mndandanda omangidwa pa nkhaniyi, and chondidabwisa mwa ena amene ali kumbali yolamulawa anasokoneza nawo and zawakhuza koma palibe olo ndimmodzi yemwe anathawira kumbali yolamula wamangidwapo mpaka lero, ndiye transparencey yo ili pati pamenepa? Bwanji osangomanga onse kuti nkhani isakule?

 11. kamlepo nkanyama kanjiso, anakanika kuchita manage kachipanipani kake kaja ka MDP, walawako u MP munthawi ya mrs cashgate banda, aziliza chitoliro kuti president atule pasi udindo wakhuta #mbohori kapena wakochedwa ndi a ulad musa, kupimpii kuli mbuzi zokhazokha zawanthu, #machende yambakatayambakata mbolo zanuzo jololo kumaima pachulu ku pitala atule pasi udindo munamuikapo ndinu,munavotera dpp? a kamulepo kaluwa ngati mwaphya pemphani thandizo osati nyansi mukuchitazi,muuzane ku mpimpiii kwanuko kuti MWALEMBA MMADZI , 2019 ikulowaso yose mpaka mkhosi nkunenatu #DPP

  1. olemekezeka ake a kamulepowo, palibe zoti waima pachilungamo mtima wao wanu wawawa nanga si hamai anu voice vanda alikunja kwa boma, ndale za a kaluwa nzo4ira amachitookochedwa dpp sizaluza

 12. Akachoka azalamula ndani anthu achambanu?poti makona onse omwe mukabera ndi kamlepo kaya mumati kamlepi adaseka basi mwadana nayo ana aulesi inu mutu ngati dzira

 13. Musanamizidwe kuti olo wina atatenga mpandowo ngakhalele Kamulepoyo kuti ndiye zinthu zisintha ata wina aliyense akakhalapo amapanga za mimba yake basi(tizingochedwa izi zinalembedwa kale za masiku osiliza anthu azakhala ozikonda okha)

 14. Yes kamlepo stands on the trueth look at peter’s face,crearly shows that he’s angry with the trueth.I,as anti DPP I say mutharika is abig thief. why is he failing to fire the ministers concerned with cashgate?.Such aperson should not be revoted.we are ready to tie him to apole and take the government.

 15. Ngakhale omwe anaba Ndalamawo atazibweza times 100 mnzanga osaukafe Palibe chathu tinali chonchi ndalama zisanabedwe,mmene zabedwa tili chimodzimodzi, tatiyeni tidzingopempha Mulungu atipatse mvula yabwino tikolole tidzikhuta zikakhala kaya muti za (basket) Kkkkkkkkkkk kaya chani, ndi zaka anthu olemela ngakhale mutakhala mubanso ngati anthu akuba ndi bible (In Jesus name) mumpeza walemela ndiye mukanene dziko? Kamuleponso ndiye mchitsilu osamamumvela amapangila kukhuta chamba mukamamumvela muthawila nthengo

 16. mmm gyz akanakhala kt malawi inagawidwa pa wiri or pa tatu mthelad bwez enafe titasamuka kukapepha nawo malo kwinako mbamba ndthu

 17. Dzuka malawi awa ndiwo alenje okupha mmalo mokoza mw wanthu wabwinoyu mukhale ozuka inu amalawi musamapepere ngati anthu osaona mukuona komwe ziko lanthu lokondedwali limukupita.. Nyasaland nzuka iweeee3èeeiii

 18. Peturo must resign,am fed-up with,go ahead mr kamlepo(sinjenjemera)u dpp suporters wake up kwacha dzukani driver wanu akugona.kkkk

 19. Ndaona ma president koma na awawa ndid hmmmmm paekha ndichiphinjo kale m’dziko muno ndipo sindikutsutsana ndi Kamlepo, vuto lathu a malawi sititha kuona patali zikafika pachipumi mpamene mumati timkadziwa izi, dzanja lalemba ndipo ufumu wao tawuza kuti walephera. We can’t wait for more damages or another cashgate to happen. Zituleni chonde prophet Pitara muntalika.

 20. Kodi wayamba lero? Nthawi ya Muluzi amaopsyeza kuti alowa mntchire, I guess he is running out of cash, give him some he will shut-up that is the strategy used by Muluzi as well.

 21. Peter Muthalika is there and he will be there also over 2019.
  U kamulepo, do you think to be head of state is a joke? Had it been u are cleaver enough bwanji siunalamulirepo dziko la malawi? How long u have had been a politician without being head of the state? Fuc off kaluwa. DPP still there over 2019

 22. am not a DDP fan koma zimenezi mungomuonelera Peter ekhayu akanakhala achimwene ake aja bwenzi pano kamulepo ata sekeledwa apo ayi house arrest lol,its funny to say this to a leader olo ntakhala ine aaaaaa sindingasiyepansi udindo coz of one munthu Lol

 23. panya pake kamulepoyo. kodi mumamuwopa iye ngati ndani.wapangapo chani padzuko lino? pamtumbo pake ngati uli ufiti ndi kwawo.

 24. Kodi mbuli imeneyi akuituma ndani?? Akakhuta soya pieces uko atikwane ife mxiiiiiiiiii,, ndikakupeza iwe ukuzitcha kamlepo uona.

 25. Cheer, cheer, cheer,,,,,,,,! I sustain the fact frm my uncle. Ignorancy tend to fool most malawians, particularly frm south and centre of the nation! We do fail to contrast ‘wrong’ and ‘right’. Blindly Loyal malawians,,,,,,! Clappng hands only to encourage 1 to squander,,,,

 26. Politics Aside , Pls Mr Prezident Wen Talking Note Dat Ur Listeners R Milions So Avoid Blanders . Y Am Saying So Has Also Given U 24hrs If He Releases D Names Of 7 Cabinet Ministers Involved To Fire & Arest Dem Or U Must Resign If U Fail To Do So! Here Kamlepo Is Tough Wat R U Going To Say Or Do? Antaba Avuwa Kaunda Advise D President Wat D Next Step ! Oyherwise Whose Going To Shut~up? So

 27. Anthunu mukamatukwanizana timangomvetsetsa poti ndi ndale za kumalawi -the opposition parties do not oppose to construct but to destroy again the rulling party never focus on wt oppossers r saying ati kutero awoneka opusa. Vuto lalikulu ndi lakuti mumangosamala mfundo zoyendetsera zipani zanuzo osati zoyendetsera dziko. AMalawi akuvutika bcoz of dis kind of politics timafuna titaona kusintha koma osintha zithuyo sitikumuona. Mmmh God’s intervetion is needed.

 28. Aaaaaaah kamulepo khala pheeeee uwone zomwe at achite yehova kwa pita ufumu amapereka ndi mulungu komanso amalanda uwerenge malemba awa daniel3vs1-,daniel4vs1-nd daniel5vs1- uwone mmene ufumu unathara wa mkulu ameneyu khala oziwa kut nzer ya chauta sifan ndi ya dziko dekha.

 29. Chitsiru Kamlepo amatero zaka zonse maluzi akamukamata. He thinks ana a Mutharika ali ngati Muluzi woti azimupatsa ndalama cholinga asamachite phokoso pazinthu za ziii. Anya awona kape amenewu boma lake ndiye si la DPP.

 30. The main issue here is not the President to resign…it is for him to take full responsibility of the current state of the affairs in his govt..including the crooked ministers he has been shielding. The president has failed us many times and in many ways. If he cant come out in the open with the names of the crooked officials then that will be his admission of guilty…and he must step down….and the current vice president will take us forward to 2019 when the masses will decide through a ballot box.

  It is so surprising that APM is fast becoming more powerful than the people who put him in power…let alone his NEC of the DPP which ought to have ellected him as the president of the party (as per democratic processes). Amalawi…tatiyeni tidzuke. This is our own country and for sure i know we love it. APM has no choice but to do one of the two things KK has asked for…either name and fire the crooks…or appoint KK as AG or ACB Chief. Most Malawian politicians are merciless with a rotten reputation. Enough is enough. The long arm of law will definately catch up with you. We have seen the cleverest fall.

 31. You Cant Talk Of Democracy In Malawi Without Kamlepo Enanu Ndi Ana Amakanda Simukudziwa How Kamlepo Influenced Malawians To Vote For Multiparty

 32. Kodi Dipp Mukutilowetsa Kuti Tsopano???.Koma Dzikolakwathu Ifeeeh.Zowona Kumangolunana Basi Chitukuko Chomangolonjedzedwa Dzakankumapita.Mmmmmh Kaya Tsipano.

 33. We r in democratic govt, 1000s of pple, excluding kamlepo,voted 4 dis president. Dont wory kamlepo osaona kucedwa wait 2019 u’ll win after u vote 4 ur self & some of ur family mambers

 34. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkk, yeah,you have provoked more than Commander, you were just passing by.Please dont take drugs when stepping podium, addressing the [email protected] take care of your speech,Kamlepo is innocent, please stop intimidating people, doesnt you know the proper logistic of approach, in such cases.by the way who are you.in parliament we have different committees and those are the responsible people that he could inquire from. And the very Kamlepo is in Public Finincing Committee.Again the president can inquire from Auditor General.this is high time now,our politicians should stop covering wrong actions,and being fond of propagandas.If i were the President i would have checked the advisors and embrance the same PAC to work with to know the truth.Our tax payers money isnt accountable,we are rich we are not poor in malawi, but we have bad leader

 35. akamulepo akanangonena ngat akufuna kulamula dzko lino.km mbwelela zawozo ndye apeze wina omuuza anali kt pamene ndalama zinkabedwa bwinotu nayexa timufufuza

 36. Tell me which country limene munthu m’modzi wa opposition anauza the ruling president kuti atule pansi udindo nkuthekadi?….koma Kamlepo…kkkkk

 37. ambiri omwe mukususana ndi bigman kamlepo ndinu zimbuli mapeto mudazolowera inde bwana zilizonse pachichewa pali mawu oti usi sufuka popanda moto. sinkhani za ku dadwe izi zomwe mumanamiza ana kuti nyau zimadya ziwala alekeni uzindikira ayankhule zomwe ndi za size yawo

 38. iwe kamlepo ciyambile ndalezako cifukwa ciani umakonda kuzuzula olamulila kodi iweyo mavuto omwe ali dziko muno iweyo ungawakwanise kaya ndi fodya wamkulu mawu amenewo suwomuza mtsogoleli wanu kaya mumaganiza kuti ungalamulile dziko izo ndiye uyiwale mwaiwe mulungo sanawonemo usogoleli munalibe ndipo iwe si idi amin

 39. Anyone who is against kamlepo statement is not just a fool but a complete mad person. You cry foul of cashgate but when someone says the truth you pull up tribe cards. We will not tolerate stupid imbeciles to be taking Malawi backwards. We don’t denounce peter coz he is your uncle but the asshole running the country. So for the better Malawi, DPP has failed!!

  1. kkkkkkk,, Wakwithu nyirenda ukuwaputa anthu kkkkk taona zimenezi ndi chani abale,,, Iweyo nyirenda sunabepo ???…. Ithink ndiwe chitsiru kwambiri tikamakuuzani kutu agalu inu simuzalamula dzikoli u think we are joking… kkkkk …. keep dreaming… kkkkkk..

 40. iwe kamlepo ciyambile ndalezako cifukwa ciani umakonda kuzuzula olamulila kodi iweyo mavuto omwe ali dziko muno iweyo ungawakwanise kaya ndi fodya wamkulu mawu amenewo suwomuza mtsogoleli wanu kay

 41. You brainless idiot so called kamulepo washota eti kkkkk boma lake siiri kuti ukati fwifwi akupasa ndalama walemba madzi galu iwe.osangopita kokunja unarikunja bwanji kod bushiri unja sanakuchulere eti.kamulepo udzanenapo zazeru koma galu iwe.ndikuona akafuna kukumenya pamaliro Amai ako chifukwa chosanganiza galu iwe koma wandikwana bwanji.inu gayz agalu enawa akupanga support kamulepo ndianja aimikidwa mtchito inu anja amagwira tchito mwachinyengo.anthu gayz ankhara minyezi osalandila anthu akuba chifukwa chake kulira kwachuluka.kip it Mr President afwinyeni ndintthu agalu amenewa we need to sweat for sweet

 42. komabe timva mene zingakhalile kumalawiko ibu rest in peace mukutibela kwambili . kapumeni musakakamile zinayamba chochitu kwakulu anu aja samalani

 43. Atsogoleri athu a ku Malawi, bwanji kukonda zokokanakokana??? Just in mfundo zanu zabwinozo kwa Prezident and share with him. Dziwani kuti mwina tsiku lina mudzakhala inu ngati mungathe kutero mu nthawiyo.

  1. It’s too late for that. There is no need to discuss. If you caught stealing you are prosecuted and jailed. So the same law should work on them

 44. Lets be realistic. Can really a democratically elected head of state simply resign just because some opposition politician has demanded so? Can someone give me one example of such rare cases please? Bring us real sound ideas that could bring in some rays of hope. There was time when the late Dr. Bingu had tough times in parliament, he had no MPs or he had few when he ditched the sponsor party UDF, there was impeachment thing and so tough situations for Bingu, that’s the time some of us thought the president was going to resign. Did he? Another example is president Jacob Zuma of RSA, he is currently not popular, some calling him to step down. Has he? Give us mature topics to argue and debate rather than trying to catch the media’s attention by uttering useless statement of which everyone including Kamulepo himself knows that it can’t happen!

 45. Kamulepo akunena zoona kodi amalawi mzazuka liti? Ndiwakuba amene komaso ananenakuti iye alibe prbm ndiopusa ameneyo.

 46. READING MOST COMMENTS IT SEEMS MOST OF U ARE UNDER 18YEARS AND U HV NEVER VOTED. JUST WAIT IN 2019, MUKAMAZAVOTA KOYAMBA.. PLIS ZAPITENI KOVOTA MU UNYINJI WANU KUTI MUSAZANONG’ONEZE BONDO IFE TITAWINITSA WATHUWATHU MUTHARIKA…. ZAWERENGENINSO MY COMMENT…

 47. This moron think he is making any sense by his shameless stances. If he is wise and not a caward let him say the names basi. No hide and seek. He shud not waste our time with attention seeking and sympathy. Malawians refuse to be disturbed by such nonsense. And its unfortunate peter will remain ur president until 2019 and there is nothing u can do about it..

 48. Kodi Kamlepo Ndiye Ndaninso? Akulephera Anthu Enieni Amaudindo Awo Odziwika Bwino Kumupangitsa Resign President Iyeyu Wangodya Khobwe Uko Nkumatero? Kaya Mwinadi Zitheka Pajatu Kachepa Tsonga Mtima Unga Phiri.

 49. These people r mad in their minds they r calling for resigning while they have done nothing to show that they can help our mother malawi to grow up

 50. am i getting this right ? #munthalika gives #kamlepo 24hrs to give out names of the 7 minister indulged in the cash gate scandal. and then #kamlepo gives #munthalika 24hrs to resign. which means #munthalika is on the list ( head of the snake ) thats why #kamlepo is calling out #munthalika to resign.

 51. Vuto lovota ndilimenero,thus y enafe zovotazi njee!..kuvotera munthu kuti azikuberani,kumalemera inuyo umphawi nkumachulukirachulukira! kkkkkkk tulo amalawi,bola kumangolimbikira kusamala banja lako,kuposa nkuti udzitaya nthawi kukakhala palaini,kudetsa chala ati ndimulemeretse Bwampini kkkkkkk

 52. Everyone wh z talking ills abwt Kamlep hz completely got it all wrong. Thnk of it, th guy z extraordinary nd courageous. Thnk of hw much he z risking hz life jst to speak out th views of th grassroots. I thnk Kamlep represents a true patriot, one of th rare characters tht r lacking in most, if not all, of our beloved legislators. Show some gratitude guys, th guy is fytng fo our own sakes as far as i cn see

 53. Palibe wabwino pa dziko lapansi and osazakhulupira munthu amakhumudwitsa khulupiran amene akukupasan moyo amene ndi mulungu bas azakupasan zonsowa zanu ndpo simuzakhala mukulimbana ndi andale pakut oipayo wasikira komweko bodza,umbava ndi utambwali zili komweko.Loran yesu alamulire bas

 54. Guyz nkhan ndi ya k 577 billion basi si za ndale zanuzo pano ku chipatala olo bandage kulibe ma exray anafa kale kale mmalo mokonza zimenezo mukuba ndalama oh icry my poor malawi

 55. this could be a good thing if this president step aside,our country is fully dwindled in everything from economic to the education! but still more they want to run the country into a veld .

 56. Ndatsimikidzadi kuti Kamlepo ndiwafodya, Malo mopeleka maina amatinamidza kuti ali nawo aja akukamba zina, Ukunama iwe mpaka 2019 komanso adzawina kaya wina afune olo asafune izi ndizomwe zizachitike, Kulibe chipani chotsusa chomwe chingadzapedze mpando ku Mwera, Anthu akumwera amadziwa choyenera kuchita,( mark my words )

 57. I’ve million plus reasons to forgive this headless idiot called kamlepo and his followers bcoz he who does not know, does not know that he does not know. Shame to you all sons and daughters of bitches who are waisting your time by supporting this brainless idiot for you are plying a complete loose game. Musaononge misonzi yanu yoti muzalilire 2019 pano plz. Keep your tears poti kuliku simunati.

  1. U guess with a question #wysonalistoto which school did u go?? waonetseratu unyapapi wako apa kuti umamwa madzi ometera ndebvu hehehehehehehehe

  2. Atleast Chihana did something that Malawians can remember him but this mooster is jst displying uchitsiru wake to Malawians. but its ok kut mwina zidzukulu zathu zizamveko kuti once upon a time there was a certain idiot by the name of kamlepo

  3. No need for insults buh its pretty clear that Mutharika has failed us all…..tiziti simukuona zomwe zikuchitika kapena mmene zinthu zikuyendera mudziko muno

 58. amene akunyoza kamlepowa ndi amene komanso amene makolo or ambuyawo amaba ndalama za boma. inu monga simukuwona kuti dzikoli likupita kuti??? Malawi wanga ine,,,vuto kwa ifeyo inu ma billions mumabawo akukulimbitsani mitima… nkuwona mukudana ndi chilungamo akunena amene inuyo mukuti ndi wamisala. Koma dziwani wamisala adawona nkhondo…

  1. Agalu ena sakumuziwa kamlepo, kamlepo analimbana ndi kamuzu, kubweletsa matipate kumene muli inuko. Achina Muthalika kulibeko ata giver za kumalawi. ndiye kamlepo saku lakwitsa

  2. Peter Dennis Mandevu 100% correct umaziwadi en ex solider also.vuto amalawife sanje ndi umbuli dats why timakhala busy kumayang’anila mavuto athu waiting for donors kuzatiesela dats why akunyoza Kamlepo makape enawa

  3. kkkkk.. Mtumbuka aliyense anabweretsa matipate…. mesa anayambisa chipani chake hw many of u voted for him….. chafikana kutha opanda kukhala ndi mp… olo mmodzi….. As long as amachokera ku Emchakachekeni, hewe, emanyareni… nkhozo, ndiye kuti anabweretsa matipate…. kkkkkk gulu iri kaya jini…. kaya nantongwe kkkk sirizatheka kkk…

 59. KKKKK, KOMA ABALE BWAMPINI, WABALALIKA TO STEP DOWN KAMULEPO?? KOMA ABALE ATSOGOLELI WENAWA ADZISO NDIYE KAYATU. KOMA KAMULEPO SAKUMUDZIWA ETI? AKAMUCHOTSE UDINDO MUNTHU WA CHIPANI CHINA? KUMENEKO KUTETEZA MBAVA ZAKEZO ZISAONEKELE POELA?

 60. Nthawi ya chair kamlepo amapita kusanjika kukaophyeza kt ndilowa mchire then chair amatenga thumba landalama kumpasa kamlepo atalowa bingu, anamuza kt lowa ukandipeza komweko. Atalowa aunt kett mmm akuluwa amamva kukoma mpaka kuwapasa udindo , lelo walowa peter akuluwa ayambapo matukutuku kufuna kuchuka . Manyanzi bwa??

 61. ine ndiona ngat kut apresdent athu akangotulusa mayina s anthu amene ali okhuzidwawo kut anthu aobe okha ngati akuluakuluwo alipo kapena ayi nde kuti kukhoza kukhala kophweka kwambiri kutsutsa zomwe a kaluwa akunena.koma kut aziti akaluwa atchule sizichita bwino chifukwa tiganizira kuti akunena zammutu kapena akungotchulira zidani.a presdent tangotulusani mayina ambava zonse kuti tione ngati pali anthuwa

 62. Don’t vote these greedy hyenas back into the government kick them out of power thru our votes these hungry ministers involvedin this corruption scundal

 63. Sametana,,,,,,,,atambwali,,,,,, Hon Kamulepo,,,, more powerful ,,,,,Awopa ndani anphwetsa ndi kugulura mano Mkango,,,,uyu ndi ndani uyu???

 64. mufune musafune muthalika alowa tchile basi aliyense amene Ali mbali ya muthalika ndiopuxa panya pake muthalika must face music ….iwenso kamlepo we can’t even trust mbuzi ngati iwe ndani sakukudziwa ??? nkhani yaikulu pano ndiya DPP yaononga ndipo ikupitiliza kuononga dziko a lomwe ndi achewa mukadzamuvotelanso pitala hell fire burn you

 65. Kamulepo ndidolo zamatikitiki tikitiki kkkkkkk tiye nazo wabwera boo osaopa munthu ,ndopa zako zikhala diesel iyendesera ufulu Wa democracy.

 66. gyz,,dzuka malawi yapanga post mayina ambavazo…Kamlepo is mot wrong chifukwa mpanda mano wanuyi ali pa top of the line…Anaba 240 billion….Kwatsala pang’ono kuti tiyambe civil war….Ndipo ichitika mpakauyo atule mpandowu…

  1. Only in malawi? From Rwanda to Zimbabwe to south Africa to India to Japan list goes on and on… The fact is a President is popular with his people… Straight forward

 67. ankhani omwe apezekapo pa msonkhano wanu. Dziwani kuti si a malawi onse amene ali DPP members. A Kamlepo simikizilani amalawi ife ngati cashgate yinachitikadi potchula maina aa okhuzidwa mosayang’anila chipani, udindo kaya mphamvu zomwe alinazo. Amakhoti azakuthandizilani chilungamo chanu. Zija munapangana zachinsinsi zalepheleka. A Malawi tonse tsopano tikuyang’anila kwa inuyo. Ngati mulibe umboni ingopepesanipo. Kaya ndi president kaya munthu wamba akangopezeka ndi mlanduwu amusatila Osward Lute

 68. mbuzi ya munthu kamlepo making noice for nothing. kalowe ntchile ngati zakunyasa. omwewo ankakugulira magalimoto wo. muthalika sakunjenjemera ataaa…wasuta chotsakaniza ndi aluvela et? bwinootu muzapenga akulu inu

 69. Mmm tisamunyoze kaluwa chilipo waona vuto lathu amalawi tinazolowela uphawi zoti tkubeledwa tilibe nazo chilichose mziko muno ndichodhula kma voti yanu inali yaulere plz plz plz tadzuka malawi palibe azabwele mkutikonzela dziko ndife anthu amene tkuvutika tingasintheso nyengo zathu…

 70. Ndamodzi awaaa amachita kutumana kuti adziyankhula chomchi……kuseli nda bwezi……zidzasitha zipani zotsutsa zikadzayamba kukhala ndalama zokwanira………

 71. Iyi sinkhani yandale ayi. ndi nkhani yakuba. Kulibwino a Hon. Kamlepo Kalua atchule mwatchutchu anthu amene akuwaganizira kuti anaba ndalama zaboma kusiyana nkuti alamule a president kutula ansi udindo pamene president amasankha ndi a Malawi ambiri kuzela ku mavoti. Azawachosanso ndimavoti. Apresident musamuopyeze munthu pomufunsa zinthu ndinso nkhani ya Cashgate siyosangalasila anthu. Chifukwa amene mukuwauza siziko lonse koma ndi achipanu chabe. mwamwayi ife a Malawi timamvera kuzera mwa atolank

 72. Kkkkkkkkkkkkkkkkk at Tambala walira… ngati mukungokangana nokhanokha koma u r not ruling… mpaka kuitanitsa Tate akugwilizanitsen inuso nde mbuzi zeni zen be united ngati mukufuna mdalitso olowa m’boma….. atumbilile achabechabe

 73. Zikatele zithela mommu without any action.Continue Blind folding ur own people You poor Hypocritical, theaves,mulderers,selfish politicians…… God is watching and U think without Transparency,ur dark forces and acts wont be known.hooo!!! Watch and learn.

 74. A dpp ndinu mazoba palibe chomwe mukuziwa mumalolera muzivutika mumat bola mukulamula ngat ukulamu y? Ukuvutika? Shupit anthu aba inu mukuwapopa kkkkkkkkkkkkkk ndinu anthu omvesa chisan cz mukuononga sogola laana anu

 75. Kamulepo just tell me the Names ku inbox kwanga ndiwatchule tiwone zomwe president ameneyu angachite Ife amalawi mwatimaliza kale potibera Msonkho wathu chatsalanso ndi Chani??

 76. Kamlepo ndidolo amakana zodelera first tym Mutharika gave him 24:hrs to named those 7 cashgates lero ndiyeyo akuwapatsa 24 hrs abwana president ha ha ha ha this is democrasy evryone has rights to say wat he/she wnts! panthawi yakamuzu kunalibe matama ngati amenewa kungomuloza chala kamuzu iweyo ndiwakumaula baxi

 77. Mr Kamlepo always voiceless as an empty tin. His lucky for Presidency expired and will never renewed again. Mukuti ndichifukwa amongokhala Wanganyu nthawi zonse kuti azidekha kangachepe. Anakakhala Munthu wina ndikanamukhulupilila komanso kukhalangati Wa chigawo cha kumpoto iya! Ndikukhala kwawo kutokota pazifukwa zawo. Zana federalism, lero atule pansi udindo zazii!

 78. koma ngati kamlepo umadya chamba tabwera kuno i think ukudya vubwa bwera ndizakudyetse ma kicka eni eni udzalowelele mtchire zenizeni

 79. kamlepo ngati amadya chamba ndakayika koma kamlepo wazolowera chabe kudyera boma mnjira yopusa ndiye pano atsogoleli wonse kaya ndi abusa nawo anaphya bele uyaluka kamlepo uyu ndi wina

 80. Pali amalawi omwe ali ndikhungu saona. Ndiagologolo saava. Zoona chikusalatsani ndichiyani zomwe akuchita president wanu? Inu chikhalire munayamba mwadya mbewa ndi ziwala nthawi yanjala? Kuzibisa mbava osazimanga? Kuyamba kampeni nthawi isadakwane? Basi ndadziwa mukumunyoza dala kamulepo mukufuna kuti makolo anuo asamangidwe kuti akakulipirini ndalama zomwezo ku colladge yadulayi. Koma mudziwe wamisala adaimba ng’oma ochenjera adavina. TIYE NAYONI KAMULEPO ADZIWENSO!!!!!!!!!!!!!!!!

  1. Kodi Anayambila Muja Kunyoza Atsogoleri Muja,kapeyu Ndatopa Naye,palibetu Zifukwa Zeni Zeni Zomwe Amanyozera,tsono Asamanamize Amalawi Kuti Amalankhulira Amalawi Ayi, Indtu Ayi,asiye Kulimbana Ndimtsogoleri Ngati Ali Ndi Nzeru,ndatopa Kumva Zopusa Zawozo.Chipatala, Bt.

 81. Onse amene akunena zoipa za kamlepo ndiakumwera, chifukwa? Mbuzi zimakondana mbuzi zokhazokha! Wakwiya ndi muroyi!

 82. Chisankho titakhala lero muthalika akhoza kuwina kwambili. Kamulepo adapenga kalekale nthawi ya UDF umunthu udatha ndipo amene adamuika pampando ku people’s party kamulepo samadziwa kuti ndiwopenga?

 83. Inu tangomulekani neyeso ndiufulu wake.Ngakhale wamisala aliso ndi ufulu olankhula.Awa anayamba ndikale kubwebweta zosathekazi.

 84. palibe munthu yemwe amavomela akachita choyipa koma cabwino ndiye manja m’mwamba ndikawonetsetsa athuwa akubisana kusonyeza kuti adachitila limodzi chifukwa ngati akukana kodi 577billioniyo anaba ndi abanki omwe amasungawo ngati athuwa akukana

 85. u said u hv de names why not releasing them. u r full of propaganda

 86. Mutolika Pitala,you thought Kalua will not respond. Kalua is a human being, hundsome and wise person. Pitala kunyada nkhope ngati tonde thats why maganizo ndi zoyankhula zako zonyasa. Appoint him as he is saying and if he doesnt mention after appointing him then let him rot in prision. Hope this deal with mature

 87. APM a disgrace to the nation. why can’t he be man enough and dismiss the culprits? he is supposed to be impartial. has he forgotten the oath he took?

 88. Kamlepo at it again kkkk anamupunganso Muluzi choncho mpaka kulonjeza kuti ngati atcheya sapanga resign iye alowa ntchire haha fodya lol.

 89. Beter to chau chicken here in rsa coz icant under standng u mr kamleopo. Mmmmmm ingodikila nthawi yako mdala iwe angayambe kuku lodza bwanji kodi?

 90. wamisala adaona khondo kamulepo sakunama petulo muthalika ndi azakewa ndimbala komaso amene akudana ndikamurepo pazimene wakamba akuonekaso kuti akuopa azimalume awo angamangidwe

 91. For sum of us Politics it’s not bread bt let everyone who ate some of those Billions VOMMIT them Back immediately!!! We r eatng CHISOSO bcz of these devilz. Oh My God!!!

 92. why running away from the truth you dpp hand clappers? i think you are myopic on these 7 dpp hyenas who have swindled our taxes,so please work up dpp supporters from asleep, mukuthawa chilumgamo ngati bwampiniyo pamene chilungamo mukuchiona and osanamizila ngati kamlepo ndi wamisala dzuka malawi dzuka kwacha ugoneranji wa dpp iwe tambala walira!

  1. Unayamba bwino koma kumunsiku ndikomwe waoneka kuti ndiwe mbuzi kuwauza anthu kuti adzuke ndiye adzukile mcp? Mcp manyaka a chipani ndipo ichi ndi chipani chokhacho sichinawinepo pa zisaankho mdziko muno

  2. ha ha haa zovu….zedi khoswe akakhala pa nkhate sata………?? Mcp toto pano pa Mj bavalani akapoli cha ku Central komweko, Abusa bwererani ku kachisi wa Ambuye, iwe Kamlepo khala duuu, nthawi yako idaduxatu c udzanunkhaso or even u vm lo!

  3. Pakanakhala amthu 7 pa amthu 10 oganiza ngat paul mwana mowe yotamu ndikhulupilala mkhaniyi itatha koma pot amthu ali mtulo dats y akut kamulepo wanena zamzeru wina mkumat tambala walila zaz tambala ameneyo akabangule mkachisi not zandale

  4. people you dont know tambala? mpaka akalile nchalitchi inu simumadya tambala nfimawona ngati akuti tambaka walila meaning kwacha komaso tu penapake sitikuthandizana kutukula dziko koma kulowetsa pansi munthu waba ndalama nkumambisa kodi auditor general simumamudzuwa zoti anapereka kalata ya ma minister 7 simukudziwa omwe aba ndalama za dziko kodi zoti suditor general akufusa kaye zichita ku Malawi Law Society simukudziwa ndiye mukuwombera mmanja zitizo

  5. Brian, ukudziwa chani amalawi ndi anthu opusa kwambiri. Anthu adaba ndalama zambili kwabasi, maina apatsidwa koma okumawabisa ndiye mkumakakamiza munthu wina kuti ndiye awulure nanga president yo ntchito yake ndi iti?

  6. Nfdie mmene kunachera muja ambuyanu akamuzu kwacha tembo kwacha busa opepera chakwera kwacha kuzada lit?tambla aliko pano ndi chihoho chanu chakwrlayo dats y isaid abwerere kukachisi

  7. The stupidity of malawians is that tachuluka anthu owonelela zinthu zathu zomwe ngati mpila, kubedwa kwa misonkho yathu tikuchita kudikila otsutsa boma kuti azichita pressurise justice, enafe tizizatukwana pa FB pano, dont we have the way to show president that we are concerned and angry like what UNIMA students did? We need mzika zokonda dziko lawo osati zobisala kuseri kwa zipani

  8. It is also my first time i hear some sence out of Davie Gama’s nonsense.Now he is the man i used to know.kkkkkkk

  9. KKKKK…. abog fool indeed…. tikukudziwani ndizapamtundu… olo kunazale sukulu mumawuzana kuti u r special kkkk… MUTHARIKA AZAWINANSO 2019 AMENE ZAKUNYASA SAMUKA UKAZIGULIRE MALO KU MAZAMBIKI…. NOSENSE!

  10. #mosted_Tembo never knows that there is sense on the word no-sense, i was never a partisan,not even now. Koma nsonkho womwe ndinalipila pogula toyota hiace van, umandipweteka,ndiye ndizimva kuti wina akuba misonkho zimandipweteka.

  11. Spot on Bezai Mbalazo, there are still people who think one tribe is better than the other, at the end we all children of a black man and woman of Malawi. Kamlepo is not fighting for any tribe, but cashgate for every malawian. But sad people condemn on tribe, that stinks!!

  12. Kkkkkkk koma kumenekoooooo kwiiiiyaaaaa Tambala walila kunja kusanache thats means wagwa nayo hahahahaaa akafika apa tambala ndiye kuti wakalamba aphwdwe basi

  13. Gaytusoh Gattusoh Noel SandramSandra, ukufuna uyambise zotukwana, nyooo! Wagwa nayo. All malawians are same, zoti Atumbuka, kaya ndani, kwa mako!! Takukanila ife, manyazi!!

  14. The Issue Is Kamlepo Gives Muthalika 24 Hours To Stepdown.Kamlepo Failed To Submit The Names He Was Asked For To The Contrary He Is Giving Instruction Instead Of Doing What He Was Denanded Meaning Insanity.U 2 Peter Are Insane Or U Lack Ability To Comprehend Matters Clearly.What U Have Written Is Contrary With The Story.U Seem To Be Schezophasic.

 93. Doung all thiz to waist our tym basi , dziko likutameni kuti mwayankhulako zakuti, koma kumalawi, tamawanamiza ana kuti ngakhale iweyo kamlepo sunabepo ndalama za amphawife, ife titenge attention yanu poti mukutiuza Oti anabanawo ndalama? nde ine ndikuti, mbava mubomamu ndizambili nduoi palibe chomwe mungachite, kuthetsa izi,nde osamabwera pa public ngat ndinu ma holy holy

 94. Ine ndikufuna ndikuuzeni a malawi kuti sitimatsatira chilungamo koma chuma cha munthu.mwacitsanzo ndi nkhani ya malo ku thyolo awandale amatengedwanso ngati wamisala koma lero umboni ukufuna uoneke choncho tieni tasiyile achuma azikangana okhaokha cifukwa pa mawa muzakhala zitsilu ndinu.

 95. Ma vote onse aja omwe anthu ana votela peter mutharika aja ndizoona kuti angakhale opanda tanthauzo chifukwa chamunthu m’modzi yemwe ana votela chipani choluza??? Mudikile 2019 ( siwandale ine)

 96. Kamlepo akupweteketsa anthu amene ukuwamverawo, nzakoyonso ndimwamuna payenkha. Mpando umenewo aliwo siwamasewera, ngakhale wina aliyense osusa kaya ndani ukuwadziwawo kokhako ndikumtunda amakuopa. Ndiye iwe linda madzi apite ndiye udziti ndadala, kunena kwa ndithe-ndithe nathambwe anazitengera. Nzakoyo ndiye wayamba kukuuza mau amenewa, ndiye iwenso ukubwereza mau omwewanso ai ine ndili pano,kumva ndikuona agonje ndani samala.

 97. Kamulepo mbuzi yamunthu akuona ngati ife timuthandizila za misala zakezo,,, 2019 DPP izalamulaso iweyo kamulepo uli mmene ulilimo

  1. Yes fellow country men and women let’s love our country,let’s take out the spirit of jealousy, greed and let’s feel our pockets with the spirit of patriotism. Our country is beautiful . mayiko enawa ndiolemela koma tikunena piano alone fresh water kuvutika nkhani ya madzi enieniwa;pajoni pomwepa. No matter the leader let’s learn to lv our country and the leaders at hand.ndimangoti ndilakwisepo nanenso pong’ono abale pepani ngati wins zamkhumudwitsa

 98. Mamina ali mwa chitsiru chili ku state house chakubachi chikamayenda kumayang’ana mwamba kusonyeza kuti mavuto awanthu chilibe nawo ntchito,maminawo ali mphuno mwakemo ndi mwamasopatazi ake.

 99. Kwanga Nkumangoombera Mmanja Chabwino Ndi Choipa Chomwe, Ndine Wosauka Ndilibe Mawu, Ndikhuwe Pang’ono Or Kwambiri I Wil Stil Gain The Same (nothing

 100. Koma tuu akunena zoona Peter zikolamkulila ayenela kutula pasi udindowoo ngati pali President yemwe walephela kulamula zikola Malawi ndigaluyoo pitala iyaaaa

 101. Kkkkkk, koma #Kamlepo wapenga eti? Ana a #Mutharika samaopsezeka usaziputsitse wekha. Just find out other things to do osati uzilota maloto masana

 102. The problem with this man is that he does things for show, not for the love of the pple he represent.Childish, jerousy and regionalistics politicts

 103. Aa koma yah Ine ndinkati kamulepo anachilatu koma ndikaonetsetsa misala sinathe M’mutu mwake muuzeni atisiyile Handsome Peter mpaka term yake yithe kkkk

 104. Nyansi ya munthu… Ithink atolankhani amene amajijirika ndi nkhani za mbuzi imeneyi… mukuti kamlepo….. The more u insult and disgrace mutharica the more we will show u in 2019 osayiwala majority rules. Who are u to gv head of state 24hrs to resign…. u are talking to millions of supporters who still love thevpresident.. instead of enticing them with good manners and real mfundo u are insulting him…. U must be very stupid!

  1. Iweyo ndiye chitsilu cha munthu how can you clap hands for thieves?? Malawi sazatukuka chifukwa cha ma kape ngati inuyo ndikhulipilira ndwe mulomwe paja ndinu mbuli..iweyo ukasapota peter it doesn’t mean anthu onse amamukonda

  2. Anthu ife tikuyenera kumaganiza kuti kodi Malawi akupita kuti? just imaging rate pano ili pa 53.53 ndikukambatu za rero komabe mkumamuomberabe mmanja munthalika?Amalawi tidzazindikira liti?malawi akupita kuti kodi?mpaka afanane ndi Zimbabwe? dziko langa!!!! work up Malawi work up my country

  3. Anthu ife tikuyenera kumaganiza kuti kodi Malawi akupita kuti? just imaging rate pano ili pa 53.53 ndikukambatu za rero komabe mkumamuomberabe mmanja munthalika?Amalawi tidzazindikira liti?malawi akupita kuti kodi?mpaka afanane ndi Zimbabwe? dziko langa!!!! work up Malawi work up my country

  4. Anthu ife tikuyenera kumaganiza kuti kodi Malawi akupita kuti? just imaging rate pano ili pa 53.53 ndikukambatu za rero komabe mkumamuomberabe mmanja munthalika?Amalawi tidzazindikira liti?malawi akupita kuti kodi?mpaka afanane ndi Zimbabwe? dziko langa!!!! work up Malawi work up my country

  5. Yassin, you the most stupid person more than everyone here. Chitengereni mpando Peter wapangapo chani cha nzeru? Some months ago you were dying with hungry what did mnthali do to sort out the problem? and was saying that he don’t have problems. I am not in Malawi and I will never come to stay in Malawi but when my fellow Malawians suffering I get concerned

  6. Kkkkk….. Looking @ the replies are just cousins, brothers, from the same kingdom….. Mutharika azawina with landslide victory.. Idont see any one who is ready to rule this country. What Isee is abunch of fools and idiots calling themelves Politicians…… kkkk.. And if u listen to their supporters one wonders kuti are these pple not mad… The truth pains Simon.. ndiwe omvetsa chisoni ndi amnzakowa….Ovota ndife inu Phee… There is no way Ican clap hand for afool. Ifetu timasankha pulezident thru the ballot ndipo tizachita chimodzimodzi 2019…. AMENE MUKUNYOZANU MUNAVOTERA KONGERESI, PP NDI ZINA ZIJA….. KOMA MASAPOTA A DPP PALIBE AMENE ANY OF U CAN CONVERT TO START HATING HIM THRU SUCH NOSENSE APPROACHES. NEVER!….. The more u insult Mutharika, the more his supporters stand firm……. take it or leave it…… just wait in the next 45months…….zisewerani pa facebook ovota ali kwa phweremwe, petrommora, nkhande, malaka, bangula, Neno, mpsupsu, namitambo, limbuli just to mention afew…….Kkkkkkk….. USOVENGE

  7. Kkkkk….. Looking @ the replies are just cousins, brothers, from the same kingdom….. Mutharika azawina with landslide victory.. Idont see any one who is ready to rule this country. What Isee is abunch of fools and idiots calling themelves Politicians…… kkkk.. And if u listen to their supporters one wonders kuti are these pple not mad… The truth pains Simon.. ndiwe omvetsa chisoni ndi amnzakowa….Ovota ndife inu Phee… There is no way Ican clap hand for afool. Ifetu timasankha pulezident thru the ballot ndipo tizachita chimodzimodzi 2019…. AMENE MUKUNYOZANU MUNAVOTERA KONGERESI, PP NDI ZINA ZIJA….. KOMA MASAPOTA A DPP PALIBE AMENE ANY OF U CAN CONVERT TO START HATING HIM THRU SUCH NOSENSE APPROACHES. NEVER!….. The more u insult Mutharika, the more his supporters stand firm……. take it or leave it…… just wait in the next 45months…….zisewerani pa facebook ovota ali kwa phweremwe, petrommora, nkhande, malaka, bangula, Neno, mpsupsu, namitambo, limbuli just to mention afew…….

  8. nooooo guys you all stupid bcoz u r bussy shouting nosence here intead of promoting your business,farming,familyfutures, #yassin is a rite man,don’t u know that man #kamlepo is chindere,chidude,chijawaka ,apa chikhumba makopala boma achipase icho chije waka go back to #Bakili time amati ndilowa ntchire ine sanali ameneyi kamlepo wake

  9. U ar the one supporting him not all Malawians,and kamulepo wachulutsa, 5hrs ndiyokwanila kusiya udindo apakile Majoti yu. Amd Listen Mr Yassin,2019 kuti mudzabere mudzaphedwa palibe kukunyengelelani kuti mulinali m’boma

  10. onse amene akusapota peter ndi afiti ndithu otamba ngakhele sunday. ine ndili pa mbuyo pa kamulepo achoke or afe

  11. Mbuzi yamunthu ngati Yassin sinamuonepo;iwe chabwino ndichiti chimene ukuchiona mu usogoleri wa pitala? ngati uli wamukupando ndiwe galu ndipo ulibe fundo unyanyela kumodzi ndambuye akawo 2019

  12. Ndipo Kamlepo angakambe chani chanzeru kapena chomveka? Ngati akuona kuti anthu amamufuna pa u president angodikila mavoti azasikimize kuti anthu samamufuna. Akufuna angotola Ngati ndi chinthu chopanda mwiniwake? Koma Kamlepo Ngati chili chamba sumasweka bwino kwabasi kkkkkkkkkk

  13. Ndipo Kamlepo angakambe chani chanzeru kapena chomveka? Ngati akuona kuti anthu amamufuna pa u president angodikila mavoti azasikimize kuti anthu samamufuna. Akufuna angotola Ngati ndi chinthu chopanda mwiniwake? Koma Kamlepo Ngati chili chamba sumasweka bwino kwabasi kkkkkkkkkk

  14. Malawi azayenda bwino pokha pokha anthu ngati yasini atafa bongo or kudwala misala. iyeyu kunyoza Kamulepu kamba koti Kamulepu sakuchoka chagawo chimodzi. why Muthalika is shielding corrupt officials? We want him to act against corruption in the government. ndiwe ovetsa manyazi galu

 105. Ine zanga pheee! Anga ndi maso pamene Bible likundilimbikitsa za masiku otsiliza ( Mateyu 24)………Agogo angawanso akuti,”Ukaona ntchentche zaunjikana malo amodzi,pamenepo pali zoola”

 106. Who voted for him and why? If you are satisfied, vote for him. If you are not satisfied, vote him out. That’s the power of elections but not just making noise which can lead you to nowhere, is a sign of immaturity and ignorance of democracy.

  1. Iwe ndi mbuzi ufufuzenso. Iwe opanda mtundu iwe ndindani, ziko lino kupanda alhomwe bwenzi kulibe asangalasi ngati ukuona ngati ndunama fufuza

 107. kkkkkkkkkkkkkkk Kamlepo ntima umazumza ndi a tsogoleri angati mwalimbana nawo mbuyomu? palibe chomwe timaona pa ndale zako, kwako nkunyoza komanso chitukuko ulibe m’dela lako

 108. Mathanyula sangatule pasi udindo becos he is a big thirf dzila lake lilimo mu audit report sangathe kukakhala ku thlolo kwa zicheche alhomwe ndi galu za athu pamozi ndi president wanuyo putulo nose galu

 109. kkkkk wasowa kokudya uyu! waku mpoto wozungulila mutu yi! . anazolowela zachabe, muthawi ya ATCHEYA amati akangoti ndilowa mtchire Amamunyengerela ndindalama pompo popo. koma uyu ukuputayu ndi Gayachawula ndikukayika ngati anganjenjemere nawe! uwuponda kkkkk.

  1. Apa! zikuwoneka kuti zawawa cz nda nena kuti wa ku Mpoto, komano ngati ndalakwisa Iyeyu ndi wakuti!? ngati siwa ku mpoto tiwuzeni tiziweko kwawo.

  2. Bwanji u like kunyoza Ku mpoto?iwe utchula mpoto waoneseratu umbuli wako,nkhani ndiya nzakoyo kamulepo osati mpoto,till wen uzanyoza ife osalakwa?unamvapo tanyoza pakati oro kumwera?tikuziwa kuti ndife amodzi,pls uyambe wamvesesa ndipamene uzipanga comment

  3. Thoxy Awuze amenewa… kkkk sangalamule malawi never…. They just support even zitsiru as long as ndi wa ku Hewe, Enukwenu, Emanyareni, Edigeni, Masasa, Nkhozo, kkkkkkk.. Tiye nawoni amazitenga ati ozindikira when infact its abunch of fools

 110. koma kamulepo ndioseketsa kwambiri ,akuona ngati u president amangotula ngati chitini chamadzi kuti chinali pamutu? koma chambachi inu

 111. Ngati Simuziwa Ndale.Dziwani Kuti Andale Amatukwanizana Kumbali Akumwa Tea Limozi.Ndipo Inunso Mutakhala Prezdent Mukhoza Kupanga Chimodzi Modzi.Bwanji Chatsika Wamanga Chi Manson Cha 6.5 Mgillio

 112. Musiyeni inu a opposition mwana wa mai ndi bambo Thom kwo ku Thyolo walakwa chani Pitala apa wakupasani 24 hours kuti muchule anthu amene mukuwaganizira kuti anaba ndalama za boma then inuso mukupasa 24 hours kuti apange resign koma ya ndale za ku Malawi ndizovuta kwambiri.

  1. Mmm man understand him 1st, apoint me atony general or acb boss so dat am in a better position to anounce the names, falling which resign!

 113. Kkk kamulepo iwe anati ikamafika 4utuluse squad yomwe inanjonja dola now u kom with this shit that means muthalika is a big skelem

 114. Nde kumalawi kumeneko…peter akidyera, ma supporter ali mbu, alibe kalikonso koma kuchemerera andale…za ziiii…!! Mkanali pa umphawi mpka imfa zanuuuu

  1. Idont Have Time Of Sayin Wat Ur Sayin Coz Its The Devil In You Which Is Forcing U To Speak Such Words Icommand That Out In Jesus Name Isay Iout!!

 115. Peter munthalika wapeleka 24hours kwa kamlepo kuti awulule maina acashgate ,kamlepo wapeleka 24hours kuti Peter munthalika atule pasi udindo koma kumeneko Malawi 26

 116. how about we take abrake???no president.luks lyk mw is too small to have apres.all these niggahs aint leaders they just hustlers.akutimalizila malawi wathuyi

 117. Ichinso ndiye chitsiru china cha munthu. Ngati pali munthu amene amatolapo kathu pa mkuluyu Kamlepo azidabwe yekha ukhoza kukhala kuti nawenso mmutu mwako muli mamina okhaokha

  1. mmmm m koma ndie mumadya zambiri za pitalayo Kamlepo amaziwa chilichonse cha MW umufuse wa mcp , Udf akuuza za Kamlepo iwe ndindani kutsutsa za munthu wamkulu