Gulewamkulu jailed for rape

198

The Dedza First Grade Magistrate court has sentenced a 19 year-old man who raped a 14 year-old girl while in Gulewamkulu regalia to 8 years in prison.

State Prosecutor Sub-Inspector Wedson Nyondo told the court that the convict, Lazaro Maxwell, and his friend were in Gulewamkulu regalia when they met the girl at a certain bush which separates Bowazulu and Kalipande villages in the district.

Lazaro Maxwell

Lazaro Maxwell jailed.

Maxwell chased after the victim and when he caught her, he forced himself on the young girl.

“The incident was reported to Chifumbwa Police that led to arrest of the suspect and was charged with an offence of defilement,” Nyondo told the court.

In court Maxwell was found guilty and Prosecutor Nyondo begged the court for a stiff punishment to the convict saying he tarnished the image of the Chewa dance.

When passing judgement Her Worship Enett Banda concurred with the prosecutor and sentenced the convict to eight years Imprisonment with Hard Labour.

Maxwell hails from Chatondeza village, Traditional Authority Chilikumwendo in Dedza district.

Share.

198 Comments

 1. Koma anthu atha mantha mpaka kugwira gulewamkulu chilombo.Pakadakhala pafupi ndikadapita kuti ndikachiwone kuti chili mu ninja (mask) ku jail ko.

 2. Koma anthu atha mantha mpaka kugwira gulewamkulu chilombo.Pakadakhala pafupi ndikadapita kuti ndikachiwone kuti chili mu ninja (mask) ku jail ko.

 3. Kkkkkkkkkkkkk mzimayi oyamamba ku Malawi kungonana KUCHINDIDWA, KUNYENGEDWA ndi chilombo pambili ya Chewa ku Dedza.
  FUNSO;
  KOMA IYEYO TSIKANAYO AMATHANDIZILA:p

 4. Ok. Gulewankulu is regalia. The 19 year old man raped underage girl. I hope Gulewankulu has no case to answer but a 19 year old man. Where was Gulewankulu when this man raped the girl? Did Gulewankulu witnessed the rape? Who ordered Gulewankulu to go with this 19 year old man? The one who ordered this Gulewankulu has the case to answer. Apart from rape, the girl was intimidated. Between the 19 year old man and Gulewankulu, who intimidated the girl?

 5. Chifukwa Choti Boma Ikulekera Kukala Ngati Gule Ali Ndi Ulamuliro Winawake Pa Anthu. Anthu Amalemekeza Mowopa Gule Wamkulu,izi Zikuyenera Kutha Now Check This Out.

 6. Chakwera woyeeee kkkkkkkkk… Za pa mtundu mukudziwana… kodi mesa guleyu amakhala nyama?…ndiye mmalo mokawedzedwa wawedza wake mkazi by force kkkkkk…. kkkkk…. Zama Card basi …..

 7. Mukuti Gulewamkulu wagwilira Mwana? Tatitathauzileni bwino bwino pamenepa kuti tikhale ndi maumboni wokwanira. Gulewamkulu sali Mugulu la anthu ndichinyama chimenecho chakuntchile zitheka bwanji kugwilirira munthu wokhala ndi anthu? Ndiye akakhala kundende ya anthu kapena iliponso ya Gulewamkulu yomwe amakhalako?

 8. awe mwandi ine zandinyasa uyu ayenera kugwira ndende moyo wake onse. (1) watipangira nkhadza ife akazi poti naise tili ndiufulu osapangidwa khadza kuchoka kwa amuna,(2) aononga mbiri ya mwambo wanthu ife a chewa ayenera agule apangepo kanthu apa ndiupuwa wachita uyu munthu

 9. uyu amangoyeserera nyau osat gule wamkulu ai inu amalawi 26 due u know gule wamkulu km? samalanii ndimalankhulidwee anuwoo,,, uyutu ndimunthu pic mwaikai sigulewamkulu mumamuziwa gule wamkulu? foolish osatiipisira our culture

 10. Are you desperate in need of watching Barclay’s premier League live matches for free, movies, wrestling and many more ????, call or whatsapp me for cheap installation on 0881687272, 0999172498 ——MAXLIN CONSULTANTS—— ——EXPERIENCE THE BEAUTY OF FREE TO AIR 4 LIFE——–

 11. Are you desperate in need of watching Barclay’s premier League live matches for free, movies, wrestling and many more ????, call or whatsapp me for cheap installation on 0881687272, 0999172498 ——MAXLIN CONSULTANTS—— ——EXPERIENCE THE BEAUTY OF FREE TO AIR 4 LIFE——–

 12. Ena atengerepo phunziro osati basi mwavalavala dzivalo zanu uko mukagwirire.Mukuganiza kuti simugwidwa ayi iwe Mnyamata sewenzani zakazo kuto musazayambirenso .Uzazindikire kuti ndichibwana zedi ukazatuluka 2024

 13. Ine ndikazangopeza mwayi olamulirako tsiku limodzi lokha ndizathetsa ine nyatsi zimenezi gule wamkulu ndiye chani? Kuthawa kulima basi mapeto ake muziti mudziko muli njala koma inu muli busy kugwirira atsikana dziko liyenda?

 14. Mlanduu ukanayimbidwa ndi akudabwe ndiamene akanaziwa chilango chilango cholangira wawoyi km acourt alephera kugamula cz chikathawa tu ichi sinanga chilombo

 15. Gulewamkulu nde chaniso mwina ukananena kuti mnyamata osalankhula ngati inali nyama, zovala povinira ukanazisiya apo ndikuyamba ndi mnyamata so so so…..

 16. we are now going to far with this, can’t u practice your culture in a right manner?….please as u are practice your culture u must also respect other people’s rights, you are a human being with a spirit, so puting on that mask doesn’t change u to be an animal, so don’t take it serious, u are nw becoming stupid with it!

 17. Mnyamatayo dzaka zake ndi zochepa pa mlingo woyenera kukwatira.Chonchonso mtsikanayu dzaka zakenso zikuoneka zochepa mafunso anga ndi awa:Mnyamatayu mukuona kuti ndioyenera kuimbidwa mlandu wogwirira ? Poti pamlingo wovomerezeka wabanja sanafike zomwe zikusonyeza kuti iyeyu ndimwana.Kodi pamenepa sizikusonyeza kuti mulanduwu ndi wa ana azaka zosakwana kulowa m’banja? Mwaziwa bwanji kuti wagwirira ndi mnyamatayu poti onsewo zikuoneka kuti ndi ana adzaka zochepa komanso omwe sanafike pokwatira/kukwatiwa? Mmaganizo anga onsewo ndi ana ndipo zomwe akapangazo sizomwe m’banja zimachitika chifukwa dzaka zawo sizikuwafikitsa ku mlingo wabanja.Amapangira zibwana poti ndi ana.lthink this case is out of constitution by looking the legal ages of marriage fr both concerned parties.

  • mr Nyson mwafunsa mfunso labwino kwambiri, choyamba muonenso kachiwiri zaka zamnyamatayu 19years-14years=5years kusonyeza kuti anasiyana ndi zaka 5,ok wamkulu ndi mnyamatayu zomwe zikuonekeratu kuti anagwiririra mwana, malamulo adziko la malawi amati munthu yemwe wakwanitsa zaka 18akuyenera kukavota pamene wa14 years sangavote Why??? ndi mwana, tivomeleze kuti mkuluyu anaphwanya ufulu wa mtsikana wa chichepere, mr Nyson musaiwalerenso kuti kugwiririra kumabwelanso motere ngati mwamugona mkanzi momuumiriza iye asakufuna kumatchedwa kugwiririra. kodi akanakhala mlongo wanu mukanamva bwanji?chilango chiperekedwe ngati achipatala avomereza kuti adamugwiririra, ine maganizo anga akutero bwana.

  • mr Nyson mwafunsa mfunso labwino kwambiri, choyamba muonenso kachiwiri zaka zamnyamatayu 19years-14years=5years kusonyeza kuti anasiyana ndi zaka 5,ok wamkulu ndi mnyamatayu zomwe zikuonekeratu kuti anagwiririra mwana, malamulo adziko la malawi amati munthu yemwe wakwanitsa zaka 18akuyenera kukavota pamene wa14 years sangavote Why??? ndi mwana, tivomeleze kuti mkuluyu anaphwanya ufulu wa mtsikana wa chichepere, mr Nyson musaiwalerenso kuti kugwiririra kumabwelanso motere ngati mwamugona mkanzi momuumiriza iye asakufuna kumatchedwa kugwiririra. kodi akanakhala mlongo wanu mukanamva bwanji?chilango chiperekedwe ngati achipatala avomereza kuti adamugwiririra, ine maganizo anga akutero bwana.

  • Zoonadi bwana mwayankha bwino.Dzaka za mkuluyo ndi zokwanira kukhaladi wamkulu maka posatengera dzaka zolowera m’banja.Chofunika tiyeni tilimbikitse ena kupewa mchitidwewu.Thanx alot.Komanso pakufunika kukhala transparency maka pa dzaka za munthu wamkazi, chifukwa zinazi zikukondera.Pena pakumakhala kunama pa dzaka zamkazi pamilandu yotereyi.

  • Mr nyson,kukondera pa zaka zilibe ntchito in this issue inuyo mungoonjezera nzeru panokha b4 shwing yur weak mind kodi nkhanitu ndiyogwirira sizimene mukuelekeza apapa

  • Munthu akakwanitsa zaka 18 ndiovomerezeka kukwatiwa kapena kukwatira koma ngati sadafike pa zaka zimenezi ndiye kuti ndi mwana. Ndipo inu mukuvomereza nyaunu mukukhala ngati mukutakasa ntima wanga bwanji! Apa chilombo chagwiririra inunso mukuvomereza. Koma mukuganiza bwinobwino?

 18. Anamuziwila zikang’a kapena anasupuka chala akuvina?nyau zonse zi burn’edwe kaya ya hip hop kaya yotani.so help us ‘NYAU KILLA’lomwe

 19. Tiwuzeni Zoona Chilombo Ndichiyani Ndi Munthu Kapena Chinyama?Ngati Ndi Munthu Mmatchulilanji Chilombo Kuti Chagwirira Mtsikana.Kukhotetsa Nkhani Bwanji.

 20. Ufulu Waanthu Ndiochepa Kusiyana Ndi Nyama. Nanga Nyama 8yrs Koma Akanakhala Munthu Mukanamva 14. Equasion Imene Munagwilisa Ntchito Popeza Zaka Za Nyamai Tiuzen

 21. Zosayenda, munthu akagwilira 14 years in jail pamene chilombo chikagwilira only 8 years, which means anthufe ufulu wathu n’gochepa pano pa dziko?

 22. Zosayenda, munthu akagwilira 14 years in jail pamene chilombo chikagwilira only 8 years, which means anthufe ufulu wathu n’gochepa pano pa dziko?

 23. Kkkkkkkk am sure kuti anthuwa ankadziwana bwino mene pena amaonekera muja agalu amenewa sakanakwanitsa kumuchita point kuti ndi uyuyu ai kkkk sexxy gule ,ma overstay anamupweteka heavy!

 24. Ndepalinso zinyau zina zikumaima munseu kumaimisa magalimoto nkumapempa ndalama, wina ndaameneyu wagwilirayu mmmmmh it’s too much now let’s unite as malawians and burn them!!

 25. My name is Monica Philp and this a testimony of how i became HIV NEGATIVE, i have been suffering from HIV for the past seven years, i have spend a lot of money finding cure for HIV/AIDS until i found this true man who cured me completely with his powerful herbal medicine, i have tried different means to get this virus out of my body, all the possible ways i tried did not work out for me, i came across doctor olumo through some amazing testimonies concerning how Dr Olumo has cured different people from various kind of sickness like HERPES,HIV/AIDS, CANCER, with the help of his powerful Herbal Medicine, so i was encourage and i contacted Dr Olumo i told him about my Sickness, He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with Dr Olumo he finally prepared for me the herbal medicine which he sent to me through courier service and he also gave me prescriptions on how to use it, after taking the Herbal medicine for some days, i went for test to confirm and the result was totally negative ,i went for test again in a different hospital still the same negative , Today i am fit and healthy to live life again, I am so happy for the good work of Dr Olumo in my life, if you are having a simillar problem kindly email HIM on { [email protected]} OR CONTACT HIM WITH HIS NUMBER OR CHAT WITH HIM ON (WHATSAPP) (+2348138956767)

 26. hey wat a fuck!…… yu mr admn , u sayd its gule wamkulu hu has raped yet yur also sayng 19 year old man, hu has been jailed gule wamkulu or 19 year old man?

 27. Shame!! kuipitsa mbiri ya chikhalidwe…let others with same wicked minds of turnishing the image of our culture learn from this