Musadye zitete: Malawians warned to keep away from ‘locusts’


locusts

Following a spate of attacks by a swarm of locusts in the Lower Shire Valley, Malawians have been warned to keep away from the insects that are being sold as a delicacy in some parts of Malawi.

In a media announcement that was monitored by Malawi24, Illovo Sugar Company who have also been affected by the disaster of locusts have advised the Malawian public to not consume insects that are being sold in some parts of the country.

“We applied some chemicals to kill them as they had invaded our sugarcane plants, as a result most of them have died,” a spokesperson for the company was quoted as saying.

locusts
Locusts have struck the Lower Shire (Google image)

According to Illovo, there is a high chance that some of the locusts being sold in the market are the ones that they killed after they invaded their field. Such insects have been said to contain harmful poison which can in turn kill people.

“We are advising the Police in the roadblocks to confiscate any insects that are being transported from the Lower Shire valley area,” said the Illovo PR.

Last month state President Peter Mutharika was accused of telling Malawians that they should be eating insects as a way of beating the hunger situation in the country. Government spokesperson Patricia Kaliati said that the President was only joking on the issue.

178 thoughts on “Musadye zitete: Malawians warned to keep away from ‘locusts’

  1. Like facebook.com/nyasascandol and Enjoy the Rest of your Life. Musalore 2016 athe Musanapeze achikondi through page yathu. Like Like Like

  2. Ife tadya kale ndipo sitikuonaponso vuto olo wezi,Nasimango tandipaseko madzi ndimwere.mulungu wayanka basi,no wonder mphalabungo zinasowa pakatipa now i see chifukwa chake kkkkk

  3. Komaso ife sitisiya kudya mesa analamula ndi gwape wanuyo ndelelo mukut tisayelekeze zimapha zapha ndan tiwonesenitu nanga mitembo yake ngat anthu akufa ndekut akupha ndi piter wanuyo zakhutu bas

  4. #apa tinve ziti a president akuti tizidya zitete inu mukuti tisadye zitete, mukutizunguza nanzo mutu ife mukhale pansi mukambilane kuti mutiuze chimodzi

  5. Zidyewe Zimenezi Guyz, Anatiuza Kale Kuti Titha Kumadya Akatundu Amenewa. Atamwalileyo Ndekuti Watopa Nkupuma. Mulungu Wapeleka Zidibwe Basi. Tisadye? Mwapenga Eti?

  6. Zitete ndi big deal mu L-city.Tikumwera Tea zimenezi.A president ananena okha kuti tidye zimenezi becoz its like MANA from Heaven.

  7. kkkk bt dziko langa Inu!!!!! thawi ya kudalibe sugar, yamayi kudali bonya nw dzitete kjkkkkkk nanga atabweleyo mukuganiza adzabwela ndichani? kkkk

  8. Mr president you must do something.illovo sugar company is trying ur patience.Why are they poisoning your God given zitete?…

  9. President wamaso mphenya Peter adaziwiratu kuti zikubwera tizidya ndiye inu osutsa president mukuti tisamadye ndikukanena kuti mukuletsa kudya zitete

  10. Kkkkkk apereka zitete zija eti mmaona ngati zizipezeka ku Admarc, nanga mbewa or makoswe bwa? Idyani anzathu akummwera, president wanu adakulangizani kale!

  11. chomwe chamangidwa padziko lapansi kumwambanso chizamangidwa ndie ngati anati muzidya zitete ndie mulungu wabwelesa zitete mukutinso musadye kkk

  12. Thanks God You still Share Malawians something to Survive on! because not all of us can afford meat or Fish. Keep on providing for your malawi

  13. Chonde amalawi anzanga a kunsanje ndi nchiwawa osadya zitete sitikuziwa kuti zikuchokera dziko liti mwina zapopoledwa mankhwara a mphavu komwe zikuchokerako kupewa kuposa kuchiza chonde moyo sagura

  14. Bwana wankulu anatiuza kuti tizitafuna zimenezi,,,,,,,,makamaka chija timachitchula kuti Mphangala,,,,,,,inu mukususana ndi a bwana ???

  15. Bwana wankulu anatiuza kuti tizitafuna zimenezi,,,,,,,,makamaka chija timachitchula kuti Mphangala,,,,,,,inu mukususana ndi a bwana ???

    1. Zidyewe Basi Guyz Zina Tikagawileko President Wanthu Amazikonda Kobasi Paja Anati Titha Kumadyako Zamchilezi. Mulungu Wadalisa Atafe Nazoyo Ndekuti Wangotopa Ndikupuma.

  16. Ndetizidyanji pamenepa munthu wankulu anati izi ndendiwo sikuti anango tchu ayi ndikumene ana choka asana fike pomapa tsidwa ulemu asana chitole chikwama zinali ndiwo zake zimenezi nde zitete lol

  17. Muzitigayila ndiwo inu aboma kodi? Ine zitete sindingasiye until i will die. Ndipo ndiye momwemo zikukomelamo eeeesh

  18. Amati mtengo wopanda zipaso munthu sanga gendemo ndi mwala iposo kalikonse kwa prof APM ngakhale konama kakang’o no yimakhara nyimbo ya siku ndi siku amutola nkhani athu,so far thr is real something visionalable 4 the beterment of our country from the state president

  19. Amati mtengo wopanda zipaso munthu sanga gendemo ndi mwala iposo kalikonse kwa prof APM ngakhale konama kakang’o no yimakhara nyimbo ya siku ndi siku amutola nkhani athu,so far thr is real something visionalable 4 the beterment of our country from the state president

  20. Mukut tisadye ????? Phwanya yokoma ngat omenei tiphwanya zimenez ndimafupa omwe zabwela zokha miracle zitete kkkkkkkkkkkkk

  21. Why not…ithougt Mr President..Proff Arthur peter advised us to go for them…they ar delicious & more of vitamns…if u wana to differ wt me…hey drop ur digits muone..muzivere nokha

  22. Posachedwapa mwalankhula kuti anthu azidya zitete popewa njala lero mukuti anthu asadye zitete, ndiye timvere ziti tsopano?

Comments are closed.

Discover more from Malawi 24

Subscribe now to keep reading and get access to the full archive.

Continue reading