MCP members order Chakwera to leave the Party

Advertisement
MCP leaders
MCP leaders
MCP leaders want Chakwera out.

He left the Church to take over the oldest political party in the country. Now the people whom he found in the party wants him to leave the party and maybe return to the Church or wherever he can fit in.

Malawi Congress Party (MCP) president Lazarus Chakwera is facing fresh calls to resign as the party’s leader, this time from some of the party’s long serving regional and district committee members.

The members organised a press conference on Wednesday in Lilongwe where they demanded the resignation of the party president for failing to unite the MCP.

Over the past few months, divisions have been rocking the MCP with some members accusing Chakwera of being behind the disputes and of sidelining some executive committee members.

Lazarus Chakwera
Chakwera faces an uproar.

The MCP officials at the press conference also levelled similar accusations against the part leader saying they have lost confidence in Chakwera’s leadership and they want a convention to elect a new leader.

“You hear one problem after another in the party. We do not have a leader in MCP who should deal with the problems,” said one of the officials Chatinkha Chidzanja Nkhoma who is believed to be eyeing the MCP presidency.

Meanwhile, MCP spokesperson Jessie Kabwila said it would be a good idea if Chakwera’s predecessor John Tembo mediates over the wrangles in the party.

She added that the mediation would be necessary now since 2019 elections are just around the corner and the party would need to be united ahead of the polls.

Kabwila who is a legislator has also faced persecution within the party. Recently, she was chased away from a Chakwera rally in Salima together with another Member of Parliament Felix Jumbe.

Advertisement

278 Comments

 1. Have you ever read 1 Peter verse 17 . I think you have not read it because if you have ever read it you would respect the former presidents

 2. MCP ili ndi maoffice sapangira press conference ku Lodge – walipira ndani nanga anatani kupita ku HQ ngati ali a MCP genuine.

 3. Onsewa akunena za chakwera ndiotumidwa ndi chipani cha DPP ,cholinga chosokoneza chipani cha mcp,chifukwa ndichomwe akuchiopa?pa MBC napo ayikapo anthu otumidwa okhaokha ,?ndiliti a MBC anayikapo za mcp pa tv,?za umbava basi

 4. Zandiopsa ine anthu abanj limodzi kuwonesan zikwanje,wat more tikazalamulira? Matsiku omalizadi mtundu ndi mtundu uzaukilana Dats it.

 5. Chakwela ndi deal sugenda mumtengo momwe mulibe mango DPP ikunjenjemera,komaso inu mukuweruxa chakwela kamba kaubusa inuyo ndiye ochimwitsaso kuposaso iyeyo ena Ainu simunalarikepo ngakhale kwa munthu mmodzi iyeyu ndibusa paka lero muyambe mwalapa zija ZANU mkumakamba za iye oweruza ndi Mulungu bax osati inu,mumakonda mdima kuposa kuunika kuwala kukadza mdima umathawa opa iyeyu MCP ingakhale chani chakwela is a leader not bwampini wazitete uja mukufuna muziba bwino eti

 6. ndale zinayambila mu mpingo so chakwela nayenso ndimunthu musiyeni achilamule chipani inu muzingodya ndalama mwalandilazo mbc mpaka kutengapo mbali zawonekelatu kuti simulinokha kumamukusokonezela chipani chifukwa chazofuna zanu bwanji simukufotokoza chifukwa chenicheni basi ngati zakuvuta yambani chanu chipani

 7. ndale zinayambila mu mpingo so chakwela nayenso ndimunthu musiyeni achilamule chipani inu muzingodya ndalama mwalandilazo mbc mpaka kutengapo mbali zawonekelatu kuti simulinokha kumamukusokonezela chipani chifukwa chazofuna zanu bwanji simukufotokoza chifukwa chenicheni basi ngati zakuvuta yambani chanu chipani

 8. me2 ndikulimba coz of chakwela atadzaluza. pita asadzapezeke mudziko muno pita ndimuthu oyipa kuyambila khope nanji mtima nde manyimanyi i love chakwela ngati momwe ndimadzikondela poxayiwala kudya deyile tangowona ka smile kachakwela evn muthu oxamudziwa yekha amadziwa kuti khopetu izi ndizawulamulilo iwe chakwela tadikila ndingomuvula peter 2019 ndidzakuvale iweeeeeyoooooo mcp nde kudya kwa ine khope za dpp zofumbwa zokhazokha izi nde zichani???zopuxa dpp?muchoke inu

 9. me2 ndikulimba coz of chakwela atadzaluza. pita asadzapezeke mudziko muno pita ndimuthu oyipa kuyambila khope nanji mtima nde manyimanyi i love chakwela ngati momwe ndimadzikondela poxayiwala kudya deyile tangowona ka smile kachakwela evn muthu oxamudziwa yekha amadziwa kuti khopetu izi ndizawulamulilo iwe chakwela tadikila ndingomuvula peter 2019 ndidzakuvale iweeeeeyoooooo mcp nde kudya kwa ine khope za dpp zofumbwa zokhazokha izi nde zichani???zopuxa dpp?muchoke inu

 10. Ine kungochoka chakwera nane ndisiya kusapota MCP…chifukwa chiyan mukulimbana ndichakwera nthaw zonse,chakwera nd munthu osalakwa,sindikuona bvuto munthu kuchoka kumpingo ndikuyamba ndale…

 11. Haha koma seriously if MCP is really serious of going back into the government then they need a strong leader not Chakwera ..sindine wandale ndimaganizo anga chabe

 12. God can’t support evil propaganda raging from hatred and those propelling this shud know that their own doom is just around the corner, they cannot win this battle . Chakwera is Mcp legitimate leader whom u can chase only thru barrot at the convention at a rightful time not being forced by the disgruntled group without a name but though it can happen today they will come frustrated again becoz pple will still vote for him. Three is nobody among them who can compete with him and be mcp leader.

 13. chakwela ngwadyera sangasunge chipani anga adachila aJZU Tembo!nkona akukamira nyumba yampingo.kodi sanvankukhu ngati emeyu adzalamulira bwanji dziko?poti akulu adati khalidwe liyambira pa nyumba.if he fells to manage MCP What about a country!!!!!!

 14. Koma zilikoliko ku MCP ko ife a DPP tili pheeee kudya ma dollars. Hahahahahah Chakwera uyisova bola kumakangolandira chachikhumi kwa a kristu bas.

 15. Muchedwa A Dpp Mmalo Mot Muzimufotokonzera Uyo Peter Zinthu Zomwe Zikumvuta Mdziko Muno Mungolimbana Ndi Dr Chakwela Amenewa Mantha Chan? Mwagwa Nayotu Coz Pano Chakwele Ali Mmaganizo Awina Aliyense Mudziwe Zimenez

 16. If MCP want to see it through in 2019 ,then this infighting must stop @ once or else forget.Let mcp learn from its past mistakes bcoz john tembo and chakwamba failed the party because of things like this, so MCP wake up from your sleep, without doing that history is going to repeat itself, Abraham Lincoln once said “A house divided against itself can’t stand”

 17. nonsense..ur the one who give him that task..wy ignore him 4 the first time….dont u know that John Chilembwe was a reverend????

 18. Am nt an MCP fan bt that press conference was a joke, jst two people whinning for bein booted out of the party useless people actually we don’t even knw hu they r, then MBC broadcast that becoz of wat exctally? I hav never seen them showin us nsokhano wa bwinobwino wa MCP pa news b4.

 19. Cheap propaganda from opponents. He is a serious threat to the throne. Watch out your footsteps. Chakwera the most possible presidential candidates come 2019. Boma in waiting

 20. Zoodziwika nzakuti munthu ukachoka pamaso pa yehova umapeza tsoka, Utsogoleli umene tikuudziwawu ndiwosiyana kutali ndi utsogoleli umene anawusiya otsogolela mpingo wa yehova.Ngati pali ganizo limeneli ndikuwona kuti ndibwino.Koma dziwani ichi anthu ambiri panopa anayika kwambiri maganizo awo pa chipani cha MCP chawutsogoleli wake,ngati achokadi chakwela MCP aaaaaaa mbola forever

 21. Nonse mukulimbana apa dziwami kut onse awa andale amadziwana,ndipo ife ngati anthu adzikomo isanafike nthawi yoti timvote iwo amakhala atasankhana kale kut uyu adzakhale tsogoleri…Choncho ndkungotaya nthawi chabe kumalimba kut eee Chakwera eee ndani a DPP mungutaya nthawi,mother Malawi wll still stand…

 22. It is clear that those who have non performers as leaders clearly know that they have numbered days and they must sleeplessly think of the only winner of the 2019 elections

 23. Zikukubowa zako izo, koma abusawa tidawauza kale kuti, bwelerani ku kachisi, so if you compare him to pope, solomon, david, zusiyana kwambiri coz this one is chakwera.

 24. That Fox Shud Endeed Leave The Party Immediately! Timaona Ngat Mwna Pot Achoka Ku Zamlungu Atha Kumatimvera Chison But Ummh,he Is Also A Greedy Maggot!! Muthamangiseni Ameneo.

 25. zitsiru zimenezi,mwadya za dpp kuti muzilimbana ndi Dr laz.manyazi mulibe. ine wanga ndi chakwera yemweyo mpaka yesu azabwera.

 26. a DPP tamadyani ziwala akupatsani ku lower shire zo….mulungu ndiwachikondi ndipo ananenadi zoona kut mwana sangapemphe nsomba kwa atate ake ndikumupatsa njoka, apa zaonetseratu kut mulungu wapereka zomwe anapempha bwampini

 27. Zaziii!!!! m’malo moonetsa mpira wa tnm obwereza muli buzy kulimbana mchipani chotsutsa mbc tv pano bwenzi ikusangalatsa amalawi poonetsa ma pologalam abwino ngati mpira game ya bullets ndi silver manoma ndi mafco siver ndi blue eagles moyale ndi redlions,ma film osati daily za dzipani mkesa chisankho chidachitika dpp idapambana lero muli busy kuchita kampeni dikirani ukuchekani mpeniwo?????

 28. It’s very unfortunate that the main opposition party should be in such squables as we move towards the next general elections. But basically, when a church leader abandons the flock and opt for politics, those are clear signs of loss of direction and beginning of confusion. People leave politics and go into the religious endevours not vice~versa. May be Chakwera should go back to the church!

 29. Kwa onse otsatira chipani cha Mcp komaso Chakwera musatekeseke ameneyo ndinamondwe amene afuna kukugwetsani koma inuyo muimebe, muona chipambano chake, tikuyamikaso nonse amene mukumunenera zoipa Chakwera mukugwira ntchito yabwino ndinu amene mukukweza utsogoleri wake, pajatu anthu anamunyoza Nowa kuti wapenga pamene iye amawauza kut nthawi yatha tiseme chombo, samkadziwa kut akukankhira kutsogolo, mmoyo mwanga ndikuva kukoma ndikamaona komaso kuva zotere. Zimene zikusonyeza kut Mulungu wava kulira kwaanthu kut lisero lomwe likupeta lero likupetera mbali imodzi, kummwera kokha basi, Mulungu akufuna lisero lomwe liime pakat kupetera kosekose, mulungu watopa ndikuva zoti 577bilion yabedwa, 24bilion yabedwa pamene ena akugona ndinjala, the Lord is now angrly with this kind of selfishness, tisatope kupemhera kwa amene tikupemphera kut Mulungu achotse mbavazi zomwe zimaikirana kumbuyo zikatibera ndalama.

 30. I hate chakwela ,jb,ulad mussa,kamlepo,peter, bt l like Kamuzu Chwambo,mark Kasonga I respect HESTINGS KAMUZU BANDA ,BINGU ,BAKILI but onething l wil remain wa DPP 4reva chakwela l dnt c any leadership in u iwe ndi yona uli mmimba mwa msomba shame 2 u and ur 4lowers.

 31. Kkkkkkk tikhalanaye chakwela posachedwapa kkkkkk peter watsekula kale ziseko ndiunduna amupasaaaaaa DPP woooooyeeeee

 32. Let them fight so as to reduce votes..we are here to see coz we are still poor and not even single rulling party brought us change in our villeges we are still sturving to the extent of sleeping on floor.The pains grows day by day when our members of parliament stood and say whatever i speak represents the poor in the villege …one wonders how would a villeger ask his or her member of parliament to ask government to give him a loan for him or her to buy a luxoulious car …..we are here to see u fight fight fight the winner will take the throne

 33. I hv jst finish reading the comments bt ayayayaya! #Chakwera wl never resighn” pipo ar stll supporting him as a leader of MCP! zaubusa mkunenawo simungamuweluze ndinuyo iyai kuweluza kuli mwambuye: by the way I dnt see any 1 who cn be the leader of this party than Chakwera: stop doing your nosence pls we need someone who is innocent as him… give him a chance akalephera mpamene muzizanchosa

 34. Guyz atolankhani ntchto yao nd kudziwitsa dzko mmene zinthu zhkuyendera ndae sizoona kut tikhale pano tiziwatukwana ayi si boh bwanj ngat sunakondwe nazo kungokhala quite.

 35. The MCP as a political party belongs to malawians and not to old useless guards.The founder of MCP ,is late Orton Edgar Ching’oli Chirwa,who handed over the presidency to Kamuzu in august 1959.Today noone owns MCP,the party belongs to malawians.If you are not happy with Chakwera ,form your party or join Dpp Thieves.

 36. Kamangodyani mbewazo ndiziwala inu anthu opanda tsogolo! Kuyambira Kamuzu mpaka Bingu palibe president or mmodzi wachitukuko koma ziphwisi basi.Zoona nkumavotera anthu ngati awa akuthandizani chiyani amalawi opusa inu nkhutukumve akolokotingo ana mudya madeya inu!!!Mxiiii!

 37. I’m not apolitician and I’m not belong to any party…komano ngati zipani zotsutsa boma ngati sidzigwirizana DPP idzingodutsa mosavuta..

 38. Fools will comment negatives against Chakwera as if he is the only person involved on politics with a background of church. Mbuli inu; all life is church or you are idiots! Do you know that Pope runs the whole Vatican as a nation? Do you know David, Solomon et al; ruled as politicians their nation was full of milk and honey? Dpp tricks will completely fail you have failed, how ignorant are you people to condem Chakwera just because He is from church background? Poor subjective and upsidedown full of evil and jelous will never assist you. This Dpp is a rotten bunch of mafias full of corruption and God will for sure remove it from the mantle come 2019: God removed your Ngwazi chingamukanike ndi chiyani apapa apa? Too corrupt and shielding corrupt ministers means the whole Dpp is corrupt and yet some fools are foolishly clinging to it.

  1. Mr Binnwell you are caliing your friends fools but remember when pointing someone with one finger the four fingers remain pointing you, that is to mean that you are four times foolish than your friends

  2. My comment was not personal and some people like Noel Amin, Dizzy food, Robert Robert are attacking me personally as if they are DPP. Let me inform you I commented about DPP not you and I don’t need your comments unless if you are a party called DPP. So its wise for you not to read my comments because I don’t know you and I don’t intend to. Enanuso mungowonetseratu kuti you are the frustrared let me inform you time is coming soon that you will curse the day you became DPP members because evil is always defeated by God’s success. True to it whether you like it or not Bingu was not aware that he will die the he did and started exalting himself ljke a lusting entity. This is the way how you DPP blind members are treating your Peter Mutharika who has no vision, he snubs Chancellor College graduation and opted to roam around Lilongwe roads, his wife is beatifying round abouts yet hlspitals have no drugs. Lachifote layandikira just pray kuti mudzakhale mutatembenuka otherwise you will all perish with him. Si zitete zija mwapatsidwa? Mawu amalenga akulengelani zitete zatsala ndi mbewa, just get ready!:

  3. frustrated ppo metioning God quoting bible verses then insults others kkkkk by the way .ihave a littlest knowledge on when vatican became a nation ,,,there i rest my case

  4. Mwina muvetsetsa n’kalankhula cha makolo, o Binnwell mwati zitsiru tipereka ndemanga zotsutsana no Chakwera komabe potiloza ndi chala chimodzi zala zanu zinayi zikuloza inuy kuti ndi chitsirukwete choposa kanai,mbale nkhani wawerengayi ndikudziwa sudaimvetse mwina poti ili mchizungu. Poyamba Yalemba nkhaniyi ndi page ya Malawi 24 werenga pamwambapo pageyi siya Dpp ndipo ndi page yodana ndi Dpp. Kachiwiri nkhani akukamba akuti mamembala a Mcp akufuna Chakwera Achoke Mu Mcp. Mau wolankhulidwa agwira omwe adalankhulidwa ndi mamembala enieni a Mcp ngati a Chatinkha Chidzanja ndi Jersy Kabwira amaudindo odziwika osati inuyo bwana poti mumatsegula gate la ku mpanda kwa Chakwera ndiye kutukwana kwambiri komanso pomaliza nkhaniyi mukawerengetse a bwana anu mzere uliwonse akafika polemba mau oti D P P, ndiye mupitilize kutukwanaku koma akapanda kupeza mau a D P P mbale uyambe kudzivera chisoni kuti misala yako yochepa ija yayamba kukula pafunika madongosolo a ku Zomba Mental Hospital bwana.

  5. Bravo@ #Binwell..!!!!.. Tell them that even Joseph son of Jacob who was sold to Egypt kumeneko He later became the Governor and helped King Pharaoh…… So why being scared by one man! The Dpp knows that people out there hav seen failures performed and wickedness been exposed….. They wanted to take Malawians for granted just because they managed to rig elections by hacking Election Counting System and change figures for them to claim victory ..They are so scared of the MCP and Chakwera knowing it’s the only stronger opposition party against them… Leave Chakwera alone ! He never sook permission from anyone when he was vying into politics and not even one contacted to advise him that he should quit politics. … Osaopa !

  6. Ena ndi omvetsa chisoni, find out vatican is a sovereign state headed by the pontif the Pope. Ignorance is a dangerous poverty, subjective poverty that is:

  7. Ena ndi omvetsa chisoni, find out vatican is a sovereign state headed by the pontif the Pope. Ignorance is a dangerous poverty, subjective poverty that is:

 39. Otembereredwa uyu amkaziti opemphera osadziwa ife maso mphenya ake ali ku maufumu akudziko,aise Chakwera taonatu lero ndi izi nde pamenepa utani ? Oooo basi ndaganiza kalowe chipana cha UP chija chidaimila u pulezident malemu bingu wa mutharika 1999

 40. ZA MCP SIZIWULUTSIDWA PA MBC TV. AWOWO SI A MCP MULOER MULORE~ MUKANE MUKANE. IF GOD SAY YES DR. LAZA ONE AND ONLY WILL BE THERE, IF SAY NO TIDZAVOMEREZA NDITHU.

 41. A dpp mwachepa with your so called propaganda. I’ve never seen Mbc broadcasting Mcp press conference @ Mcp headquater before. How come now your busy with mcp. Know that people in rural areas have nothing to do with media. Those of us who follow the media, we r civilised and we all know that DPP is scared with MCP. Whats wrong with Salima???? Always Jumbe!Jumbe and his followers? Your just young todlers in politics! Mukuwerenga mmadzi. Olo mutayitanitsa convention lero Chakwera will still more win. Dpp if your serious with politics, just change some of your bad policies.

  1. conference ija a dpp yawasangalatsa kwambiri chifukwa mpungwepungwe uli ku mcp ukuwachitila campaign a dpp , inenso zandidabwitsa mbc tv full coverage

  2. Kungoti dpp yikuonjeza kwabasi. Akufuna mcp yithenso ngat udf. Amene mukusapota dpp apa mukuonetsaratu umbuli wanu inu daily pa mbc nkhan ndiya mcp. Kulimbana nayo basi. Mudziwe kut mukamalimbana ndi munthutu mpamene amatchuka. Komanso nkhani ili apa siyomatukwanana. Umenewo ndi umbuli.

 42. Zipani zizatha ngati makatani,, masiku omalizatu amenewo,, kuzakhala chipani chimozi,,,, DPPtu imeneyo,, azalumana mapilikanilo okhaokha,,, MCPtu imeneyo,, azakalowa chipani cha adani awo,,,, UDFtu imeneyo,,, azasala ma MP atatu kuchipani chawo,,,, PPtu imeneyo,, Masiku osiliza ano.

 43. Chakwera is a good leader ndipo zipani zambiri zikumuopa pa 2019. ngat pali vuto kambilanani mu mcp umo coz kwa ineyo Chakwera is a right man to be a president not peter.

 44. Nonse mukulalamuka apa ndi a Dpp timakudziwani, mukulowelera bwanji as mnyumba mwa eni ake? Mmmm chitani manyazi, osamakangodya zitete ndi mbewa akupezeranizo bwanji? Zilipo zambiri ku chikwawa, zoonadi Mulungu amapereka chomwe munthu wapempha, m’malo mopempha chimanga? Ndangodabwa nazo, Neba panga zako ana akufa ndi njala uchedwa ndi za eni

  1. Inuyo mukamakangana mnyumba mwanumo mumatitchulilanji ifeyo kuti ndi amene tikupangisa? Mukaotchelana galimoto mumati ndi ifeyo, mukafuna kuchosa president wanu mumati ndi ifeyo,,, ndiye wantopola pamenepa ndi ndani???

 45. mwayamba mmene timayamba kukhululukira pang’opang’ono mwayambapo kodi mulibe maso anzanu pa kenya mpompa akulamulabe inu basi yanu ija kaya muziona zisusani azanu akusinkha ndiwo kkkkkk

 46. I realy support this revolution.We cant win with this poer obsessed man.He rebelled against Nkhoma synod bcoz he didn’t see possibility of life top cleric.
  Politics is not his side palowe wina even atakhala Munlo.

 47. kķkķk ngati akumuukira chonçho açhewa okha kuti achoke munthuyi ndi mbuzi nañga ili mitunďu yonse munthuyudi alibe tsogolo pa ndale sadźalamulira malawi zamukulira ñdi mkhwidzi mkaduķa basi

 48. kķkķk ngati akumuukira chonçho açhewa okha kuti achoke munthuyi ndi mbuzi nañga ili mitunďu yonse munthuyudi alibe tsogolo pa ndale sadźalamulira malawi zamukulira ñdi mkhwidzi mkaduķa basi

 49. These people are being sent by the DPP. The fact of the matter is that the DPP is afraid of Chakwera therefore is trying to bring confusion. These splinter group is full of confusionists. Leave Dr Chakwera alone.

 50. Those of you who think Chakwera is misplaced you don’t read your bibles…were rulers non Christian?…rulers were even calling….asking from prophets of God…read your bibles don’t just carry them on Sundays..

 51. Kodi abale anga a MCP, bambo Chakwera akadawina 2014 ija ndikuyamba kulamulira. Maganizo amenewa anzeru zabwinozi mukadawatulutsa, bwanji ngati pali vuto kungolankhula nkhani yeni-yeni kuti anthu amve. Kulekana ndikuti ameneyu, asiye chipani ndikubwerera ku church, popeza inunso ndi anthu ngati iyeyo wopa mulungu. Pls musanyozetse, chipani chanu kukhala ngati sichiopa mulungu ganizani bwino polankhula timakunyadirani ndi ine nzanu.

 52. I think there is an evil spirit sponsoring these press conferences! Look at how often Jumbe is given platform on MBC TV to castigate Chakwera and now it is these so called veterans! Malawi will not develop as we are all looking at politics as a source of income. Wake up guys!c Look at how Lhomwes are sharing gove positions while sponsoring your infights!

 53. Sacks.. you can’t win anything without him, we still loves the party because of Chakwela, we don’t need you old goats, you’re the butch of the failures. you’re already in a returing zone, but you don’t want to give the athers a charse to rule the party, we need Chakwela not you..

 54. KKKKK, KOMA ABALE ZINA KUSEKETSA. PAMENE CHAKWELA AMKAIMILA CHIPANI SIMUMKADZIWA KUTI ANALI MTUMIKI WA MULUNGU??? KOMASO AMENE MUKUFUNA KUIMILA CHIPANICHI NDI ATUMIKI WA SATANA???

 55. I WATCHED THE SO CALLED PRESS CONFERENCE AND ALL I SAW IS A BUNCH OF IDIOTS BEING DECEIVED BY SOMEONE.

  And and a wise man here should ask himself: why the press conference being beamed on MBC TV if it was an issue to do with MCP? Since when?

  Look wisely and u will see some political strategy!! Confuse MCP and make way for 2019!!
  And in fact if really those idiots were sacked of their positions, then hail the one who sacked them!!

  They are not royal!!!

  1. anzao adayesera kuli obaba waja koma odalephera.wangukudya ndalamazo koma mcp ili mmagazi osati mtindalama owaninkhato.wakanika, walephera ngati onatumidywa kusokoneza chipani.ng’oo! Kwaacha! Kwaacha! Dr Laz!

 56. KODI MUKULIMBIRANA CHIYANI? UDINDO KAPENA NDALAMA? INU A MALAWI24 TATIWUZANI MOMVEKA BWINO CHIMENE CHATSITSA DZAYE. PLEASE TELL US THE REAL BONE OF CONTESTION. YOU TOLD US ABOUT THE DIVISIONS IN THE DPP WHOSE BONE OF CONTESTION WAS ALBINO KILLINGS. DO NOT KEEP US GUEESSING. CALL A SPADE A SPADE.

 57. Mr time is not over u can go back to God work,dont waste your time with the devil knw that politics is nothing but God govmt is good than of the human ,God still need u for the work u start so that u can finish it amen.

 58. mmmm something fishy here, where have they been all along, if indeed there are mcp supporters, why the party is not gaining support in their area. komanso kuwaona anthu ake ali mbuuu, aaa musatipusitsepo apa, mavuto ali paliponse even in other parties including in government but they don’t go publically.

 59. bwelelani kwa ambuye. kulibe mastress ndi ma relax okhaokha zitayeni zadziko izi. kalapeni ndikutumikila mulungu…ndalama ndisatana

 60. Vuto ilo!!!,ankafuna kulamula paza kumwamba ndi dziko lapansi,tsopano lero mulungu wakwiya nawo,kugwa m’manja mwa yehova ndi tchimo lalikulu kowopsa,mulungu adawasankha kuti amutumikile iye yekha,koma lelo,akutumikila milungu yadziko lapansi,hooooooo tsoka ilooooooooo

 61. Ukathawa ntchito ya Mulunga mabvuto amabwerapo ndi amenewa, Baibulo limanena kuti kapolo sakhala ndi Ambuye awiri kodi akamufuna nthawi yonweyo wina akumufuna kodi adzatumikira ndani? Lazaro Chakwera malemba amenewa amawadziwa koma anawanyalanyadza Yona,,Lero Mulungu wakwiya naye ndipo akakakamira adzaona zomwe anawona Yona

  1. Kodi anthu inu mawu a Mulungu sinawadziwebe? Mukutanthauza kut onse a politics ndiopembedza satana? Kodi chakwera ananenapo kut wasiya kupemphera? Komaso amene anakuuzani kut utsogoleri nditchimo ndindani? Chakwera sadagwe kumpingo coz sadalakwire church, Komaso Mulungu amakondwera ndi mtsoleri oopa, olemekeza Mulungu.

 62. mwadya zambili koma mukunama akukutumaniwo mwauze alimbane nd kuyendetsa dziko osat mcp nd chakwela mukufuna tonsefe tikhale a dpp ndinu aGALU inu et wakwana atupele nd udf yakeyo basi MFITI inu

 63. kkkkkkkkkk! nde aDPP akamati azalamulila mpaka kale nkhani zake ngati zimenezi,chipani chosutsa chachikulu mgwilizano kulibe kkkkkkk!!

 64. Ng’ombe ikazazinyera nchira ndiye kuti yatopa, Yehova amakana kumuzemba umenewo nd mkwiyo wamulungu mr Chatsika :D:);):):D;) shame

 65. Ndinakuuzani ine a Malawi azanga kuti CHAKWERA siwandale ayi koma MBUSA WA CHINYENGO mwaona zimene achita iye lero kkkkkkkkkkk

 66. Amayi osasamba Ku malalata zachakwela .mcp wil never win ,dpp is fueling the move to weaken the part.tipanga resign ambiri

 67. Nkhani yabwino sizachilendo anthu amayambana. MCP imalimbikitsa kukumana ndi kukambirana koma mukamawopseza tikudziwani kuti akutumani, mwadya zaweni ndiye mutha ngati Daza……..

 68. Ngati akuti upange resign kuchipani nde dziko udzapangidwa patangothatu tsiku, mbuzi yachakwera. Limbanani mupereke athu anu ku DPP ikazawina muzatiso yaberaso

 69. Where were these so called MCP supporters before and since the 2014 Elections? ? Since when did they realize Chakwera is not fit for the Party? .. If that being the case mmm I doubt your loyalty is poor as supporters . Angokutumani ena ake ndi tima a luvela kut mukhwefule Mcp ..Si Atupere mudamutha from UDF and now your stronger rival ndi Chakwera and the Kabwila. These are DPP ‘s propaganda just to out throw the Opposition.

  1. Inu ndi mbuzi siyani mikangano ya mcp ikhale ya mcp osamasakaniza zinthu , i think n bliv dat u hav a minimum of degree in Mbuziology

  2. For just replying to my stupid comment u have just really shown to be a major simpleton with just full of mucus in ur head…. Go behind me son of devil… Stupid.

  3. Akuti kuonetsa kuchenjera pa media…watch out. ..tonse si amaganizo ngati anuwo!! Ngat fb mwayiyamba kumene nde mwacedwa nazo zonyozazo! Mukadakhala anzeru mukadaturutsa matured backing points against my views!

  4. Ndiye ngati zili chocho DPP ndi madolo ndipo ndale amazitha, komaso ndiye kuti MCP anthu ake ndi opepela coz sangamalolele kusokoneza chipani chawo coz of DPP, 2019 idakali patali musaope ayi.

  5. Am not afraid as if iam a follower of any of ur parties… These are my views as a citizen. In doing so we must be careful we might drag back to a one Party State.. Of which we can’t accept in this age.

  6. Chosangalatsa yapa nchakuti A Chakwera mmene amayamba za ndale anthu analipo ….bwanji osamulangiza that time?….. Pano adalowa ndale monga mwa ufulu wawo as a citizen and I doubt if someone can convince him to drop politics and make a return to the Altar. …

  7. mmmm chipanda chakwelayo mcp ikadakhala 50 /50 wt dpp? mukuganiza kuti nduchani chidapangitsa achinyamatafe kuvotela mcp? mukamapanga ziganizo zanu zopusazo muyambe mwakhala pansi ndikuona chomwe chidakoka anthu .I thought we wnt to change things bt u guy u ar th one pulling us dawn. thnk wt hw many voter dd u loose wt en hw many wl u going to loose 2019.gv us good reasons of taking him out…nonsense

 70. Mkhristu wakugwa,koma kulimbana ndi za dziko si dhilu,kugwa mmanja mwa Yehova ndi koopsa,suja ankati Yehova wandituma kuti ndi lamulire dziko la Malawi?Nanga lero ndichani ichi?Munthu wa Mulungu kusochera nkhalango ya uchimo

  1. Read your bible again. The administration of the government used to be in the hands of men of God achina Eli & it is going back to them.

  2. Za boza politics is a dirty game that involves stealing, lies, killing, sono mu ufumu wa mulungu mulibe zimenezo osamasewera ndi mulungu

  3. Mr Chris! Upatula kut nkhani tikukambiranayi ndiyandale koma ngat mukufuna kudziwa bible mukhoza kundiuza ndikuphuzitseni, ine sindifuna kut anthu azipanga msintaplt bible, mukhale osadziwa zinazo koma bible mulidziwe, utsogoleri ndikuchoka pamaso pa Mulungu ndizosiana, Mulungu amafunaso atsogoleri oopa Mulungu, mukhoza kundipeza pa watsap on 0882731689 Ambuye akudalitseni.

  4. Chakwera Is Not A Backslider! He Is A Man Of God!! Iwe Sumadziwa Kv Munthu Angapange Ndale Opanda Kuchimwa? Ingolimbikirani Kupemphera Basi Kut Mukalowe Kumwamba.

 71. Bwera kuno kuno ku DPP axe CHAKWERA.That party is outdated,it won’t win.Ino si nthawi yomachedwa ndi zinthu zopanda tsogolo ng@ zimezo.Ona inenso ndidatayapo nthawi yanga pachabe kumeneko koma pano ayi ndithu ndidadziwa chinthu ndi chimzake.

 72. Are you looking for a powerful, Witch? Here is PROFF SAHA the Witch, after years of successful casts. i have has all the experience needed to understand how I can help you with your unique situation. I analyses your situation and help you. Are you really looking for a spell caster who can sort all your problems? Tell me about your situation.
  Regardless of your background and beliefs, the ancient art of witchcraft embraces you. Once you open your heart and mind to this awesome power, miraculous changes in your life could bring you instant love and happiness!
  CONTACT +27733947689

Comments are closed.