Chakwera meets with UNIMA students: says Fees must fall

Advertisement
Lazarus Chakwera

Opposition Malawi Congress Party leader Lazarus Chakwera has joined the chorus of University of Malawi students and other commentators in advocating for the fall of the University of Malawi fees which were raised to a minimum of 400,000.

In a media interview Chakwera who is also a Member of Parliament and campaigned vigorously against the hike of fees in Secondary Schools said that he had met with the University student leaders who had briefed him on the situation.

Lazarus Chakwera
Chakwera wants UNIMA to rescind fees hike decision.

According to media reports, Chakwera and other MCP stalwarts met the student leaders in Lilongwe where they had a brief meeting over the University impasse.

Chakwera has been quoted as saying that he does not agree with the fee hike as it is a way of defeating the investment that the country ought to make in its young people.

The meeting will most likely court controversy in the eyes of the ruling Democratic Progressive Party (DPP) who claimed that the University students have been protesting the fee hike on orders from opposition elements.

Recently, a car belonging to former Chancellor College lecturer Jessie Kabwila was allegedly petrol bombed in what she claimed was an attempt on her life for being suspected by the ruling party to have been behind the demonstrations.

Advertisement

326 Comments

 1. A chakwera mmmmmm,koma zoona Munthu kumakhala busy ndi Othawa Mulungu ? uyu moyo wake ulipakulemera, mutha kuona kuti wathawa Mumpingo kamba koti mumpingomo makobili mulibe oti angabe, koma mudziko akuona kuti adzaba koopsa. Koma tsopano chipani chimene wakwera mbili yake inada kale, palibe aliyense amene sadziwa , Man festal , a MCP . Kukhala pa chipanichi , ndimphamvu ya uchitsiru. Ndiwina ati: kwaaacha ! Kkkkkkkk hahahaha, iwe kuche kangati ?Eee! Koma tsopano wafika pena Ugalu.

 2. Enawa paja ndi ntchito amalipilidwa ndi pitala mwezi uliwonse pano musadabwe amasekelera ndi zopusa zomwe mufa imfa yowawa kodi akukondwa ndi angati nanga akulira ndi angati ?

 3. Take over Chakwera we need wise leadership not zankutu za zii, tiona ngati 2019 atabelenso makape amenewa mudyeletu 2019 mcp on the driving seat

 4. So true not everyone is a minister or MP’s child. You have the money but not our Malawian salary can manage to pay fees for university studies. They can afford to send there kids out of Malawi but ordinary people can not manage the hike here. Be realistic.

 5. So true not everyone is a minister or MP’s child. You have the money but not our Malawian salary can manage to pay fees for university studies. They can afford to send there kids out of Malawi but ordinary people can not manage the hike here. Be realistic.

 6. Good leader should address this in parliament not going to students bcoz he is not in the ruling government so he will yield nothing than seeking attention that’s why I don’t vote bcoz all leaders post 1994 are clueless what they know is insulting one another no constrctive ideas on how to build the country.

 7. Manyasa amadziwa zinthu ziwiri basi-FREE or SUBSIDY and ali ndi CHIWANDA chotsabweza ngongole lol ,HOLY GHOST FIRE! kkkkk.

 8. kkkkkk nonse amene wapereka ndemanga zanu ai zikomo.ine yanga ndikhawa achakwera pepani kwambiri ubusa unja munangowona kusia bwerelani nsanga kubusa khosa zikukudikikani inutu simuzawina olo kaya kodi muli inu mukulamula mungatani pa za fees ine chomwe ndikuona apa achakwera kkkkkkk iiiii ai inu ndiwoseketsa koma a dpp tatsisakoni fees mene kwacha akusoweramu tikalimatu apa kwaine ndingoti alemekezeke wamwambao

 9. KAYA ine sindingapange chibwana chovotera munthu, iye azinona koma ine ndilimbu kutuwa ndiumphawi, pano ndili ndi zaka 28 chiyambire sindinavote ndi sindizavota mpaka kale chifukwa phindu kwa munthu ovota palibe, timapereka misonkho mmaboda podusa kutani koma anthu amaunduna kumangoba basi nde kuti cha ? Za uchitsiru basi Fuck off

 10. Tsopano, munthu ofuna kuthandiza mukam’menyenso ndiye akuthandiza ? Inu mukufuna kuti boma litsise school fees , koma muli busy kutukwana Muthalika kumunyonza kutani, nde mukuganiza kuti zingakuthandizeni ? Mukanakambirana ndi boma mwamtendere osati kupanga zipolowe . Nde ngati mukudziwa kuti Chakwera alindimphamvu kuposa Amuthalika Omwe ndi boma, muzeni asise fees.Nonse amene muli under chakwera mutu yanu sikugwira ntchito, chifukwa Chakwera si President Wa Dziko ndi munthu wogalukira Mulungu, komanso pamutu pa Chakwera sipagwira ntchito. Now , siyani kutukwana Muthalika yemwe ndi boma nde kambirana ndiiye , akunthandizani. Koma mukatengera za chamba azingokuthirani utsi ngati mbewa kuuna.

 11. Ana Asukulu ngati fees itasike mutipangirenso ife anthu Akumudzi kuno chifundo cholipempha Boma kuti atsitsenso VAT ngakhale kuchotsa kumene pa zinthu zofunika ngati Ufa,Soap,Sugar ndi Zina zotere.Thank you in advance.

 12. first there is need for the university management to justify why they have raised the fees. a breakdown analysis of wat is needed. per student, and let the opposers also justify why the fee must go down without politics attached to it. the fees can still remain at K400 thousand and those students that cannot meet the fees then can get loan to subsidize their fee, but chanco management must be challenged to improve the high education standards so that it meets with current development demands. Its. useless to have educated pipo on papers just bcoz they passed substandard syllabuses. imagane computer programmer still uses pascal langauge in this modern world.

 13. Evans mavango, ulingatiine sindimavota zawusilu ,kuyikamunthu pabwino kenaka kusandukakapolo fuck kayazanuzo kamavotani as aresult nkhondo yilipafupi ndapitaine

 14. Ndibwino kusiya phazi kusiyana ndi mlomo a Chakwera akanakhala anzeru akanasiya phazi, mlomowu, mlomowu,mlomo udzawapeza.Mbusa wabwino amabweletsa nkhosa pamodzi osati kuzibalalitsa.

 15. Komatu zinazi ndibwino tiziyamba taganiza bwino tisanazilankhure. Ndizomvetsa chisoni ndinso manyazi kumuona munthu wophunzira wa nzeru zake. Akutenga mchenga ndikuuwaza mu pweya kuti anthu ena asakwanitse kuona chabwino chomwe chikubwera mu mlena lenga. Kutukwana ku singakonze chilichonse.

 16. Fees Itsike.Popanda Apo Ulendo Uwu Tikupitawu Chanco Tikatentha Yose.Umve Zimenezi Peter Mthalika.

 17. Those who are writing rubbish against Chakwera and MCP are real fools who don’t follow current affairs and politics. Wasn’t it Felix Jumbe who moved the moved the motion against fee hikes in secondary schools and public universities? Weren’t the fees in public secondary schools reverted to old ones after government had already ordered the ministry of education of the adjustment? Make research before writing your nonsense and showing your ignorance to others. Opposition role in a democratic govervement is to give constructive advises to the ruling party. They don’t make and implement policies, its govervement that does. So think before uttering your nonsense!!

 18. Palibe yemwe amafuna kuponda manyi omwe adapondapo kale. He was supposed to choose another party or opening his own political party not black kokoliliko he is really Mad Man.

 19. Man philip Mawaya, ana opemphapemphawa atipwetekesa mutu ndawona, koma ndingomva chisoni kuti sakudziwa kuti chakwera kungowina monga mwadzina lache zinthu zizakwera kooooopsa kopsa kujatu, koma mbuzi zimenezi zivuta kuti zimvetsetse, aaaa, shatapu.

 20. Hahahaha man Joseph ,auzeni azadeweza anazolowera eko kwaya kkkk bwera utenge hahahaha zany a mule Fuck, who is chakwera I don’t even want to hear this name 4the rest of my life, not because of his name only but also his political party is Fuck kkkkkkkk, mmmmmm , tiyenazoni ovota inu mulipaukaidi oyendera koma simudziwa, + mukavota iye ndikuwina tea amamwa yekha inuuuu ! Tamagalamukani sha !

 21. ngakhale kuti mumunyoze chakwela ndiye kuti kusowa mzeru nokha osawona ulamulilo wa peter m’mene akuyendetsela zikumuvuta angosiya

 22. Zowona peter, Anthu andale sizinthu, mbava zenizeni za anthu .Ngati palimbali ina yauchimo imene Mulungu adzaweluze nde ndindale, KAYA poti ine chibadwire sindinavotepo, nde ena ati andiphunzitse galama, kkkkkkkk mmmmmm, wt is following me ?

 23. How can feez be raised while government officials annouced that malawi is the poorest country in the world,ithink u dont want malawians to be educated

 24. His voice is nothing,like air that brows frm east to west carring flu and etc…wise people never surport wind…They surport influence for dat wind…He is dreamng a bird without wings hw cn it fly????

 25. most commentators on this wall are fools who supports DPP blindly, they dint learn a lesson in Bingus death, amaika munthu pa udindo ndi Mulungu, even munene zoyipa bwanji za Dr Chakwera God knows his destination. its not surprising your so called professor. ignores to acknowledge ChAkweras presence in his meetings. Jelous kills and cowardice leads to easy defeat, for sure DPP will be defeated come 2019 whether one likes it or not. Truth shall prevail and Justice will one day take its course and you devils ultiMately defeated

  1. Inu zipangani za gologolo zomwezo za ma election zitayeni muzingokwiyanazo each and every election. Eniwake owina ndi dpp zinazi zipani zimabwela pa back. 2019 mukuilota apayi ndi landslide ya dpp, Analiponso wina ankanena kuti anamuika ndi mulungu anaiwala kuti anavoteledwa ndi anthu oikonda dpp. Anaima payekha zinamuonekela pano angoyendayenda kunjako ngati maskin. Uyunso mukuti lazalo yudasi Iscariot palibe chanzelu chomwe akupangapo azaziona 2019 azaleka kulankhula motumbwa ngati akupangilamu

  2. you Are showing that you are too ignorant as your dpp, sunaphunzirepo mmene anafera m’bale wanu uja? your ignorance and blind dpp following will harm you, sindinalembera iwe and don’t bother responding to my comments, I don’t like cowards commenting on my sayings.

  3. kufa ndi nthawi we born and die one dy. Analiponso wina ankazicha life president but he die. Olo iweyo uzafa ndithu olo uli nthakati chotani u wil die one dy ndipo yehova anakulengela imfa yako yomwe izakakusiye kuli chete. so dnt celebrate others death like ur God himself.

  4. I’ve advised. you not to respond again because you Are not Dpp and the fact that we will die. does not mean we should. not talk, your ignorance is clearly shown on your blind following of this evil DPP, ndiwe otengeka moreover useless uneducated idiot who goes for DPP because of regionalism. you even don’t know what is life, please! respond to others and leave me alone.

 26. kunamiza munthu odutsa bodza siri dziwika koma okhala naye nthawi zonse amalidziwa,apa inu a dpp mungachenjere bwanji anthu akuona ngakhale inu muipitse wina zolephela zanu mukunama chauwera si policy yake yakayendetsedwe ka boma.ngati munazikoza kuti mudzazuza anthu mwachonchi zanu izo.ana aku koleji zokambilana zaphungu anazitsata bwinobwino simungawapangire ata ndipang’ono pomwe ndipo kutkwana chakwera ndipamene mukuonetsa nkhaza zanu zonse ndi kupusa kwanu. zofooka zanu musanamizile wina zakulakani apa boma liri mmanja mwanu ndi akukoleji sakundaulira chakwera kuti atsitse fees ai koma pitala ndi boma lake mwamvetsa. mcp motomoto kwachaaaa!!! ndikupempheni anzanga a mcp osamango amvera ziri zonse zonamizila chakwera ngati iye ndi amene akulamulira dziko ndiye ayiii

 27. chakwera you’re a loser there’s nothing to believe in you! how can old person tell himself to join young ones instead of helping to solve the problem? grow up man and be a leadership.

 28. achakwera munathawa ubusa kumapanga ndale pamene anzanu akusuliya zandale kumayamba ubusa ndipo ine vote yanga suzaiona zipangani ma demo anuwo

 29. Anthu aku aphwitikizi awa,mitundu yosaziwika bwino imeneyi.mumatinyasa nayo.anthu aphuzo ngati amenewa,amakani onsamva,odzikonda,ndikhale nao analanda malo.motu yawo simakoka.

  Anthu osagonja pa zoipa awa.koma mulungu was mose aliko.

 30. u r indeed a loving father Dr Chakwera wait May 2019 ndi boma kale inu abwana mukadzangoluza tidzagawanapo dziko lino ife central region mutilamula basi enawo akalamulenso kwawo

 31. Koma panyasaland pano nde pachuluka zoliralira bwanji kkkk. tiyang’ane za Unima fees, nanga za land bill , tikakamba mavuto ena monga mzipatalamu, chakudya , malipilo apa ntchito, kusowa kwa ntchito , misonkho yangoti mbwee , the list goes on kkk. eish Ambuye alowelerepo ndithu

  1. Bola pano timadya nkhuku ndi mazila za cashgate ndimangozimva. koma awa mmmmm kuyesela kunena kuti abale yanga ikugonela akuti katenge basi ndimazila osukusa omweo kamuzu akuwafuna ndipo zinali mbava zenizeni pano zinakawabela anthu kumpingo akufuna azamalizile Cash gate

 32. ee chilungamo chimawawa chakwera ananena kale za izi mufune kapena ayi mavuto adakalipo magetsi adulaso ku capital hill cashgate names mukubisa e kayatu anthu akudwa nyika kunsanje zimayamba delo kenako mademo dzikolonse palibepo ndale apa olo mutukwane zanu muphulika muthalika alibe zeru chanco inamulephera alinduna paja akuti muzidwa zicheche , munena zenizen mpakaso msonkho pamalo eeee koma kuzisakadi timatchadi magalimoto ndiamene mwayamba kuotchawa mukusiyana bwanji ndi mcp yakaleyo lomwe belt umbuli mumaona ngati akati profesor ndimulungu mudafela dzina zangoya tifunaso maina acashgate aja pompano kupanda kutero kumsewo basi.

 33. kkkkkkkk… the honourable Pastor is trying very hard 2 advance his political mileage, he has forgotten that him and his fellow MPs have created their economic heavens while the poor students r unable 2 generate fees. As a leader he let his colleagues ask the same poor students he claimes to stand for pay loan interest on their behalf… #doublestandardsandhypocrisy.

  1. but you don’t give facts bwana #Michael, kunyoza wl never solve matters because u don’t know God’s plan on leaders ñ human race.

 34. There is no one who can allow this shit political party ( MCP) to come again in the Government, it’s full of kubera anthu nkhuku, abankha ndi mbuzi ,makhadi mkati , who can allow it to come back again, Anthu amene akufuna munthu ameneyu ,mitu yawo sigwira ntchito, mawaya ena alumpha line mmitu mwawo .

 35. Koma kusadziwa ndimatenda owopsa kobasi, iwe wekha sungawone kuti chakwera wa akoyo ali after kuhonga anthu ncholinga chozikometsa kuti akhale wabwino ? I think wangowona kukhala Ku ma high schools koma humanity sukuiziwa, fokolo zako iwe usanditaitse nthawi, Fuck off.

 36. Chikwera spoke already for Fees Hike before these Demos l guess some of us we don’t follow what is going on in our country

  1. Iwe suziwa kuti mbuli inzakoyo ikubwela poyela chifukwa ikufuna mavoti. ukuona ngati akadakhala olamula akanachita kanthu ameneyi, amalawi adapenya pano bola azilankhula enawa koma ichicho nchosathandiza. Sindikugwilizana nazo zoti fees ikwele but this guy ndi khuluku kwambili. All the politician ndiokumba dnt trust them

 37. Good,bt is he taking advantage of the situation to discredit the government or he has another plan or solution to table,for the ‘zero def’ government?

 38. Iwe uwafunse ambwiyako zambili ya MCP, mwina udakalimwana sudziwa, ndikuwonadi ndi iwe nkhanda you are still smelling sete , Fuck usatitaise sikati.

 39. Iwe uwafunse ambwiyako zambili ya MCP, mwina udakalimwana sudziwa, ndikuwonadi ndi iwe nkhanda you are still smelling sete , Fuck usatitaise sikati.

 40. Asakushishe aise, unafunsa bwino ncholinga choti udziwe chitsiru ndiiye chifukwa sanafune kukuyankha , usamudandaule ,amagwa khunyu uyu, pusi.

 41. Asakushishe aise, unafunsa bwino ncholinga choti udziwe chitsiru ndiiye chifukwa sanafune kukuyankha , usamudandaule ,amagwa khunyu uyu, pusi.

 42. Hahahaha, he is a pastor, but he did forgot his God and starting following the political issues, he thought that may be God is after political parties, he do not know that God doesn’t allow politics. Chakwekizy is really Mad Man, lool ! How you can forget Namalenga koma mbuzi imeneyi sha !

 43. Hahahaha, he is a pastor, but he did forgot his God and starting following the political issues, he thought that may be God is after political parties, he do not know that God doesn’t allow politics. Chakwekizy is really Mad Man, lool ! How you can forget Namalenga koma mbuzi imeneyi sha !

  1. Mr. Mazango, may i ask you one question please… I am not a theologian but I did part of it for four years somewhere.. one of the calamities a man of God can do is to sin against the one who called him. so my question is…Is becoming a president or a leader of a nation a sin before God???. Give me scriptures from Bible that condemns this act. thank you.. mine is proverbs 29:2. at least use RSV if at all you have one.thanks.

  2. Ndi mbuli imeneyi Kodi David sanatsogolere dziko? Ndiwe mbuli muuzimu president akaziyika yekha pampando ndi choncho amaluza direction osankhidwa ndi mulungu samasowa amampasa dzeru thats wy anakana kulumbira ndi Bible

  1. Anything wrong bro? u are famous in that ….. Mind u chakwera is not welknown to people lk me.if u believe/trust him u will be thrown in his pit.

 44. I can see a bright vision inside this leader as he enhance to mobilise the #Feesmustfallcampaign.
  Any country without enough graduates don’t rise up from her economic chains.
  How can a poor student from a disadvantaged family manage those big funds?
  Politicians as President such asMPS and Ministers kids will be only called Graduates in Malawi
  #Feesmustfallcampaign continues.

 45. JOIN THE GREAT ILLUMINATI BROTHER HOOD TODAY AND LIVE A BETTER AND HAPPY LIFE. WELCOME TO THE GREAT TEMPLE OF RICHES AND FAME. Are you a business, Man, politician, musical, student and you want to be rich, powerful and be famous in life. You can achieve your dreams by being a member of the Great illuminati brother hood. With this all your dreams and heart desire can be fully accomplish, if you really want to be a member of the great illuminati brother hood, contact or whatsapp the Lord illuminati now, +2349052645181Note: newly recruited members are entitled with $1,600,000, A Golden Ring and free visa to United State Of America . Please will do not share blood. this is very real

 46. JOIN THE GREAT ILLUMINATI BROTHER HOOD TODAY AND LIVE A BETTER AND HAPPY LIFE. WELCOME TO THE GREAT TEMPLE OF RICHES AND FAME. Are you a business, Man, politician, musical, student and you want to be rich, powerful and be famous in life. You can achieve your dreams by being a member of the Great illuminati brother hood. With this all your dreams and heart desire can be fully accomplish, if you really want to be a member of the great illuminati brother hood, contact or whatsapp the Lord illuminati now, +2349052645181Note: newly recruited members are entitled with $1,600,000, A Golden Ring and free visa to United State Of America . Please will do not share blood. this is very real

 47. Please lets not politise this issue because we are suffering on this hike if you feel u want change anything do not involve urself we are angry we want to go back to our classes….

 48. Chakwera anatsutsa kale zimenezo, koma vuto ndi boma lanulo silifuna kuva zonena za anthu ena, to be a DPP supporter should not make you deaf ok

 49. Zingavute zingatani chakwera sadzawina 2019 ,he was there 2014 he failed ,pano for sure u have no chance again am mcp supporter from Mchinji T/A Zulu koma ife palibe will be opposers forever ,we should not bother for ourselves ,it was 2014 wen we cud hav won the elections .tikunama .tilakhule zonyasa zotani za bwampini wil never overcome him

  1. Tell him to hold the elections today and you will see. God is God. Just join the blue camp if you want since you are this hopeless. We will teach dpp a lesson in 2019

  2. Tell him to hold the elections today and you will see. God is God. Just join the blue camp if you want since you are this hopeless. We will teach dpp a lesson in 2019

  3. Hahahahahah why didnt we teach them during the last two elections,hahahaha hope the DPP will use the same mechanisms they used last time to defeat us kkkklklk Mr its DPPz time wait 2024

  4. Hahahahahah why didnt we teach them during the last two elections,hahahaha hope the DPP will use the same mechanisms they used last time to defeat us kkkklklk Mr its DPPz time wait 2024

  5. Hahahahahah teach a lesoon on wat? kkkkkkk go and draw your plan again otherwise muzalilanso kuti akibelani. Anthu mumakamila ntunda opanda madzi, mcp no mp/khansala ku south only one mp ku north how could u except to win presidential election, ndimangokumvanitu mukukuwakuwa zopanda pake

  6. nkhan isagwere kumaelectionz coz malawianz owez vote 4 munthu coz ndiwakwao nt hs knowledge on politics thts y win or loose chakwera wl owez b against stupid staff as long az politics n malawians r concerned

  7. Tionge are u sure? Hahahahahahaha maloto chabe awo inu kodi DPP yapanga zingati zosasangalatsa anthu chakwera yo ndi north nf central ili pompo komano mkuwina?

 50. Kodi akuluakulu kkkkkkkk hahahaha, kodi chakwera nde ndaninso m’ malawi muno ? Kodi iyenso afuna akhale ngati mwana wasukulu ? Ooo ! Akupanga ngati iye wabwino ? uyu nde Mayazi , lool ! Who is going to vote for him ? This one is already rejected by everybody including my gogo siteni , chifukwa adawona zakuda nthawi ya MCP. He mustn’t waisting his time there is no one who can vote for him. He must continue to deceiving the people as pastor yet he is not. Tell him to stay quite and look for Other way to do , because this is not his own Business , Oky, it’s me who say so. Fuck him.

 51. Ngati fees yakwera kungosiya sukuluyo! Mowa mukuziwa kuti wakwera mtengo koma mumagula ndikumatukwana kuti mumamwera ndalama zanu ndiye mumati maphunziro aphweke ? Musova!

 52. If I were Chakwera I would join the Dpp Part not necessaliry of being happy with its rule but to transform it into human party. These Crocodiles, Lions Elephants + Anyani they always happy to see Malawians suffering & deing wth povert but a day is coming adzaona kut a Malawi si anthu opusa momwe amaganizira.

 53. U people u dnt follow discustions in pariament thats why u r giving nosence speach hr akanapanga chani munthu anayankhula kuti akweza kwambili boma silinavere

  1. olemera inu musatinyase apa ngati munaba zambiri muzidya ndalamazo basi,ndalama zanga zamisonkho mundibe fees mukweze afiti inu.fedelizm ibwere apa anyani enanu mukunya mwano, mukutitengera kumtoso ngati maliro anjoka.

 54. vuto Mr Pig Peter and his dpp have poisoned your minds,pomwe a opposition akupeleka malangizo kuboma simumavera mkungotii professor woyee mchimbulimbuli . Ku parliament a opposition akhala akuzudzula boma chifukwa chochita trim education budget. koma ai ndithu.kuchita trim education budget kukwera state house budget, pali nzeru? Ndiye wina uziti mfwe,mfwe mfwe?

 55. Koma kupusa sikwambino eti, mesa munthu yemwe zakhuza zinthu amatenga mbali ngati bwanawa zawakhuza bwanji kungotenga ndalama kuikako kuti asise fees yo bwa?

 56. Koma choti tidziwe ku parliament amatengera majority nde ngati chakwera atakana koma the rest nkuvomera obvious bill ingoyenera kudutsa so sindikuona chifukwa chomunyozera Chakwera.That time anthu amamunyoza winiko pankhani ngati imeneyi so tisadamunyo chakwera nde dziwani majority ku parliament ndi aphungu olamula bcs number yao ndiyochuluka kuposa osutsa boma

 57. kkk poti amalawi ambili ugonthu pomwe chakwela ankafusa boma zakukwera kwa fees paja mudali kuti?kodi paja chizungu amalawi ambilife sitimachiva eti mwangodana nae chakwelayo. kkk nde simunatitu mulimmadzi

  1. Ali mmadzi ndani? kkkkkkk koma iwe munthu wake ndiye kukhala yudasi othawa kusogolela nkhosi zauzimuyi! umuuze akuchepa kwambili akalambila komweko, akuti kugula mavoti kkkkkkkk muikanso wina uyu term yake ikatha azawine ndi ameneyo koma nyasi iyi ndiye yalemba pamwala basi

 58. Icant trust Chakwera apa zikungoonetssa kuti ndi mbuli opanda tssogolo, iye zoti feess akweza anazidziwa bwanji osakhala pansi ndi anzinzakewo koma mkumatsogolera ma dem, chitsiru cha tsogoleri!

  1. Very stupid comment. It is people like you who are encouraging government to come up with stupid ideas. Have you ever paid fees for your relative? Did you expect this government to listen to Chakwera? Ukafunse mafunso ako opusawa iwe sunamve kuti fees yakwera? Nde udziti anamva bwanji? Stop being stupid for once. Chakwera si size yako.

  2. Very stupid comment. It is people like you who are encouraging government to come up with stupid ideas. Have you ever paid fees for your relative? Did you expect this government to listen to Chakwera? Ukafunse mafunso ako opusawa iwe sunamve kuti fees yakwera? Nde udziti anamva bwanji? Stop being stupid for once. Chakwera si size yako.

  3. fool..hv u eva paid fees or evn yakuprimary iweyo..kumangokira zlzose kumbuyo du u thnk boma la malawi likuyendetsedwa bwno..thts blind loyalty I swear..masalaries a ogwra ntchto civil servants inclusive ndiochepa zot fees sangakwanitse chonsecho tax akumadula kwambr on lito thngs eg bread..misonkho the govt cnt evn uz kupanga sponsor madents kma busy kuthandiza maproject opanda mfundo..idiots..dem tnk malawians r stl sleepng..azadabwa..iweyo go 4 aldut literancy xul @joe..mxiee mbuz

  4. Ithink ndinu amodzi mwa agalu omwe amangokuwa osadziwa chomwe akukuwa, let me tell you, am well educated man , my parents tried for their bst and ndine odzidalira together with my family. My parents tought me how to fish not to beg. Let me underline this …..”Chakwera” ngopanda nzeru, being aleader he cant wait demos and then standup talking so called nonses to us ! Anali kuti pomwe amakweza fees ? Ndizoona kuti iye samadziwa? Mind u am working and happy with my life. Iweyo munthu ukufuna nthandizo koma mkumaonongaso katundu , wina mkumakula mutu kumasekerera zopusazo shaaaa zitsiru za ana! Akuuzani chiyani munthu oti anazolowera kudya chopeleka, papersunday, zamasika!

  5. joseph if u dnt hav somting sensible 2 say u beta just keep quite oky? mxeee! kagone ndingakuphuritsepo chabe apa even ur name njala itself sugest how poor u r!! idiot! osamatengera chidan chakumtundu wakwanu kubweresa pa public issue lyk this rabishhhhh

  6. One thing iwant to remind you is that, your so called aleader ndi chipani chake all the tym amaoneka pomwe amaona kuti pali kena kake. Unamvapo kuti wayamikirapo china chili chonse dziko muno kapolo mzanuyo!? Moyo uli ngati mphika wanyemba umasokhonzera wekha ukachulukitsa uchitsiru mphika udzafuwa!

  7. joseph tazisiya zisiluzi … they dont know anything …….ana a unima amafuna akuti boma liziwaopa …… koma munthu alibe tsamba lililonse …….. munya mafana pano kwacha inagwa … zinthu zinadula ndiye osamadabwa feesyo ikamakwela ……. ndiye chakwela wanuyo angoyankhulila nchimbuli mbuli akupwetekesani

  8. joseph tazisiya zisiluzi … they dont know anything …….ana a unima amafuna akuti boma liziwaopa …… koma munthu alibe tsamba lililonse …….. munya mafana pano kwacha inagwa … zinthu zinadula ndiye osamadabwa feesyo ikamakwela ……. ndiye chakwela wanuyo angoyankhulila nchimbuli mbuli akupwetekesani

  9. kodi pitala nzeru amatenga kwa chakwera? ngati satenga kwa chakwera ndiye kuti chakwera ndi mmodzi odabwa momwe zinthu akuyendetsela pitalayu.

 59. Awa asamaone ngati ķuyendetsa boma kuli ngati kutsogolera kàchipani ka mcp mmutumo nzeru mulibemo àkuona ngati uyo akweza fees yo mmutu mzeru mulibe kuti sadziwa kuti mziko muno muli amphawi?

 60. Koma ma politicians ayayaya! Apezelapo chopangira campaign. But for sure, those who are applauding you are the already mcp die hards

 61. What Chakwela doing gives me no option….but to vote DPP again in 2019….He always there when things get wrong…nothing he is doing to the country to show how better he is..

  1. Your argument is not making sense boss! what do u mean when things go wrong? In other words you are accepting that it is wrong to rise school fees now? By the wat when was the last time things were right since DPP started ruling that you wanted that Chakwera cold be there????

  2. charlie …edit your english first….then think not politically ….Chakwera is doing the most wanted job……agalu

  3. U will vote for DPP simply because u want to not because of chakwera.

   Opposition inali ita tsusa kale b4 the UNIMA council made their final decision on fees hike

  4. Does that mean is only fees hike that DPP are bad at..?there are more people suffering in this country not for fees hike…what does he doing to show his better side..?

  5. mr charlie tell me who is wrong between these two: a)The one who makes mistake..b) The one who takes longer to critisize the mistakes being made…..,…why will u vote for the one who makes mistakes other than the one who takes longer to speak out

  6. Bcoz….Chakwela is busy cleaning Muthalikas’ mess…..Instead of washing his on laundry and convincing people to vote for him 2019.

 62. Opposition busy scoring political points from desperate university students.Mr Chakwera ngati multi ndi chikondi pa Ana a sukuluwa alipilirene fees onse then we will be behind you. Ife tidaphunzira sukulu yolipira ndi a malemu Ngwazi Dr H kamuzu Banda ndipo sitimachita mademo kapena makani and the results were beneficial, and look here we are today.

 63. Awanso asatichimwitsepo apa. Mmene fees inkakwezedwa ankangoyang’ana saankayankhula kanthu. Pano chifukwa choti ana ayambapo ma demo ndiye basi enawa azibwelapo azioneka ngati abwino, zamkutu. Ndakwiya kwambili

  1. Man simumaitsata parliament. He stood his ground kuti zisachitike and it was your stupid DPP MPs udf and some useless independent Mps that voted for this nonses

  2. Gorba Mika, thats too much. Pliz withdraw yur insults. Ihav checked yur profile and it says u are a teacher at some christian school. I dont expect a teacher in a christian school to be hurling insults at yur frends like this. Is that waht yu teach to students??? Do all teachers in Malawi insult pipo like this? Its too much, and u are by definition putting the name of that school to disrepute. Are u realy a christian or you just went there to seek employment? Pliz remove yur comment its to distressing. Pipo hav opposed my comment yes but not the way uhav done

  3. Am not pro dpp, and infact dpp is the worst thing i ever want to hear in my life. Howeva am not ashamed to say i dont agree wth Chakwera’s policies. John Tembo was a critical leader of opposition, very active and lively unlike what we hav nowadays. Had it been Chakwera was really strong and had momentum, he wudnt have allowed some of the bad laws passed i.e the passing of the land bill, hiking of fees in universities, i mean, JZU wudnt hav allowed this

  4. Atsogoleri Mr Chingwalu.Mu Kumunena Mtsogolerh wachipani cha anzanu kuti “zamkutu mwakwiya naye kwambiri” and yet u want Mr Mica to withdraw his statement for expressing his view. Mmmmmm atsogoleri nanu muvomereze kt kalembedwe kanu ndikokwiyitsaso koopsa.

  5. Johnstone Kasawala, i have criticised Chakwera kuti zomwe wapanga iye ndi zamkutu ndipo ndakwiya naye kwambili. I criticised him and not insulted him. Kindly put things into perspective. And i didnt say kuti Chakwera ndi galu just as wat this friend of yours has said to me. And it is very pathetic and unfortunate that u are there backing this conduct of insulting others. Zomwe wachita Chakwera ndi za mkutu kumene ndipo ndakwiya naye according to how i feel about this fees hike. Koma sikuti iyeyu ndi galu ayi mmene anandinyozela anzako ukuwabakilawo. Tizimvesesa zinthu amalawi anzanga kutukwanana ndi umbuli waukulu komanso usaveji.

  6. anyamata inu vomerezani kuti dpp ndi chipani chomwe muli anthu ankhanza kwambiri ndipo odzikonda amakhulupilira zokamba zao ndiye zanzeru kuposa za anzao tangoganizani nkhani yambendera yapassport yadriving licence ya land bill ya fees ku University ya kukwera kwa fertilizer

  7. amene ali wa dpp sangasangalale ndi chilichonse chimene angapange achakwela chimodzimodzi mcp nkhani iyi idakambidwapo ku paliament ndipo ochakwera odaikana nkhaniyi

  8. Ine wa sine wa dpp, koma zochita za Chakwera sizimandipanga satisfy olo pang’ono. Ndine wa United Independence Party. Ndipo ngatidi iyeyu nkhaniyi adaikana mu parliament, zinatheka bwanji kuti zinavomelezedwa kuti fees ikwezedwe?

  9. Kodi Chakwera ali aphungu angati m parliament?Chakwera ndi amene akulamulira dziko? Kodi okwera pakaliyala angagwire mabuleki kapena kuimba belu? Kukhala Ndikukhala basi mukakapanda cholankhula muziti chakwera walephera kulamulira dziko ndiye? mukati wanzeru mukatanhauza kuti chakwera azidza muuza zochita? malamulo ndi fundo zonyasa adapanga ndi chakwera ndi chipani cha mcp? maiko kunyanyala chifukwa chakusakaza ndalama m boma k577 bln ndi mcp? chimene chakwera akulakwapo nchiyani pafundo zomwe a dpp amafuna kuchita akalowa m boma? Bwanji Ngati fundo zimenezi sizi bwino osakalankhula mabwana anuwo atha ukumvelani kusiyana kumazungulira kunyoza amenenso iye zikumuwawa. alankhuleni aphungu anu kuti fundo izi zikupweteka akumvelani koma kutukwana wina uchitsilu akuchita ndi wina ai osatero

  10. Michael Phiri, kumbukilani bwino kuti mmisonkhano yake yoyambilila chitangotha chisankho, Chakwera adanenesa kuti saazalola olo pang’ono kuti malamulo oiphya amalawi asavomelezedwe mpaliyamenti. Izi adayankhula ku blantyre kuno pa njamba park and i was there. The same speech adayankhula pa masintha ground, then pa katoto freedom park. Ife nkumanyadila kuti wapezeka munthu amene azitimenyela nkhondo anthu opanda mphamvufe. Mchaka cha 1998, John Tembo ngati leader of opposition adanyanyala mnyumba kuwauza aphungu ake onse kuti atulukemo. Mpaka boma lidaimisa zokambilana. A Chakwera akulephela kuwalumikizisa aphungu otsutsa kuti akhale ndi liwu limodzi. Look at wat Winiko did. Ataona kuti boma likupanga trash pankhani ya ma alubino, adanyamuka yekha kukayenda pansewu. Chakwera zonsezo amaona kumangoyang’ana. Basi ndimunthu oti waziiiii,,, amadikila kuti wina ayambise nde iye azibwelano pambuyopo of which it doesnt change anythng at all. So ine ndikudzudzula mchitidwe umenewoo. Omabisala, kumakhala chete zinthu zikamachitika, then nkumazayambano kuyankhula zitachitidwa kale. Umenewu siutsogoleri

 64. Opposition busy scoring political points from desperate university students.Mr Chakwera ngati multi ndi chikondi pa Ana a sukuluwa alipilirene fees onse then we will be behind you. Ife tidaphunzira sukuluwa yolipira ndi a male much Ngwazi Dr H kamuzu Banda ndipo sitimachita mademo kapena makani and the results were beneficial, and look here we are today.

 65. Malawi needs visionary leaders like Dr.Chakwera.Let’s joiin hands for Chakwera to wiin in 2019 for betterment of our children.

  1. Jb rule through dpp akadaima payekha sakadslamulanso malawi, ndinkona anapanga mavuvu nkuima paekha ndikugadabuka mpaka kumusiya malawi kukabisala. dpp olo kuika botolo ngati president litha kuwina kumusiya chakwela akulila kuti amubela

  2. chakwera chakwera undrr my foot he is a trsnsactional leaser and cannot be a visionàry leader at no point did he state his vision all i hear is tilowe mboma ad if ali kunja

  3. Mufune musafune DPP ikutha ulendo uno.Anthu ambiri atopa nayo.Njala ponseponse zimene kudalibe nthawi ya MCP.MCP motomoto,2019 boma mukhaula paja akuti muzidya ziwala ndi mbewa ndiye mudyadi.Kodi simudakwera pa msana pa UDF inu chipani cha UP chitakukani? Ife kwathu DPP kulibe ndipo anthu zimakhala zachilendo akamamva za DPP.Kwachaaaaaaaaa.MCP and Dr Chakwera 2019 bomaaaa kuti njala ndi corruption zikathe.Mulungu adayamba kale ukulangani osakupatsani mvula yosakwana.Mbava zachabechabe inu.@Mike Mulumbe and Mafukeni Sabilika.

  4. Iwe Bright Malemya Dpp Or Kuikapo Galu Ngati Sign Yachipani Anthu Adzaivotelaso Ife Kuno Ku Zomba Sitingavotele Mcp Nyau Zokhazokha Akang’wing’wi Achabechabe,

  5. Chimodzimodzinso kwathu kulibe DPP ndipo tiwona ngati tchimo kusapota DPP.Akapondoi okhaokha.Mu DPP muli mbava zokhazokha nchifukwa chake Mulungu akukumanani mvula.Chakudya kulbetu kwanuko pamene Central Region ndi chimanga chokha.Mukudya ziwala ndi mbewa chakachino.@Kumwenda Zyikani Willie.Kwachaaaaaa.Dr Chakwera and MCP 2019 bomaaaaaaaaaaaa!

  6. Ndani amakuuza kuti kuba ndi njala kudalibe munthawi yakamuzu? hahahahahah paja mudali wana 8t mukafunse azigogo anu osatinso makolo wanu azikunamizani kuti kunalibe bcz nao akula nthawi ya Bingu chakudya chili mbweee. mvula sanamane a dpp amana southern African country’s. kwanu ngati kulibe dpp sikuti ingalephele kupambana pachisankho ndipo yakhala ikupambana zaka zonse iweyo ukuvotela osusa. Voti ya mudzi wakwanu ilibe ndiphindu lomwe olo iweyo kukhala osavota ungochepesa nambala yoluza basi osati yowina. kwacha lelonso kudacha kalekale akutibela nkhuku ndi mazila, kumachita kutenga ikugonela ndimazila osukusa ati kamuzu akadye kkkkkkkk mumaona ngati tidaiwala 8t

  7. Kuno ku Central Region takolola kwambiri chimanga.Ndani akuwuza kuti mvulla idavuta Southern Africa yonse.Kwanuko yavuta chifukwa Mulungu afuna kukulangani chiukwa DPP yanuyo siyabwino.Kodi sipaja mudatentha office ya MEC ku Lilolngwe pothawa chilungamo? Palibe chimene ukudzIwa iweyo.Nanga nkhani ya the four mid night ministers,nkHhani ya Chasowa.nkhani ya anthu 20 adaphedwa ku Mzuzu osalakwa mwaiwala?MCP and Dr Chakwera 2019 boma.Kwachaaaaaa!@Mafuken Sobilika.

 66. Palibe Angasinthe Malawi, Bible Linaneka Kale Kt Masku Omaliza Ogula Azalira Ndpo Ogulitsa Azaymba Lokoma, Maphunzro Akuyenera Kugulidwa Modula Bac. Siineyotu Ndanena Koma Bible

 67. bro and sister sibwino kumakonza zinthu zitaonongeka ai panopa ana anawathamangisa then kumachuluka m’nzeru bwanao amadziwa kale b4 panopa katundu wakwela bwanji sakuyankhula? Bwanao sakuvutika zawo zikuyenda bwino ndipo amadziwana bwanao asayankhule angokhala chete. Anataya Bible kumafuna dale pandele palibe choonadi.

  1. Symon khalani ndi mfundo zomveka! Speech ya chakwera ya ku parliament mudaimvera koma mukati akulankhula lero zitaonongeka kale? Ambuya anu ali pampandowo samamva

 68. ngati mwatsoka mudawerengapo mbiri ya israel mtsogoleri amene mulungu samamufuna amakumana ndi milili ndiye Chakwera ndiye mtsogoleri ovomelezeka

 69. ngati mwatsoka mudawerengapo mbiri ya israel mtsogoleri amene mulungu samamufuna amakumana ndi milili ndiye Chakwera ndiye mtsogoleri ovomelezeka

 70. Not only fees but everything must fall at the market in stores bus fairs and all. If not then DPP must fall we put the into power in 2009 and they put themselves in power in 2014 but now they are bosses for themselves.

 71. Not only fees but everything must fall at the market in stores bus fairs and all. If not then DPP must fall we put the into power in 2009 and they put themselves in power in 2014 but now they are bosses for themselves.

  1. Akafa ameneyi sikuti ndi dpp yafa. Tizaika wina azalamulilanso dpp ndichipani chadziko lamalawi lili ndi aphungu ndi makhansala muzigao zonse sikuti ndi central region party only. so musamalote zoti peter atamwalila lelo ndiye kuti mcp ilamulila ai. Adaeselapo jb kupha bingu pano mzimu wake ukumusowesa ntendere akukanika kukhala kumalawi kuno .

  1. Dont trust political is there make his bright future not help. He fail to push in Parliament instead he push salary and loan ndiye mukuyembekezela usogoleli wabwino mwaiyeyo.

 72. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my deities, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before a month my body start developing my skin start coming up after 2month I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via whatsapp +2348162447651

Comments are closed.