BREAKING: KCN students protesting in Lilongwe

Advertisement
KCN Students demo

Students at the Kamuzu College of Nursing (KCN), a constituent college of the University of Malawi (Unima) are currently staging demonstrations against the recently announced fee hike in Lilongwe, Malawi24 can confirm.

The students started the demos at around 6 AM.

They blocked the road that leads to the Kamuzu Central Hospital torching tyres and forcing road users to change routes.

It was at this point that armed police officers dispersed them by throwing teargas canisters until the students all returned to their campus.

Malawi24 understands that no arrests have been made as of now.

The demos come in unison with the recent protests that happened at the Chancellor College in Zomba and the Polytechnic in Blantyre.

The University of Malawi (Unima) announced a fee hike in all its constituent colleges.

The fees see Chancellor College as the cheapest with its mature students paying K900,000. The Polytechnic comes next with a fee of K950,000.

Mature students studying at Kamuzu College of Nursing will be required to pay K1,000,000 while those at the College of Medicine will be asked to pay K1,400,000.

The students want the Council to revise this decision.

However the council has indicated it will not rescind this decision.

(more to come)

Advertisement

189 Comments

 1. Eee, asis , Sakala Bettina Marie, Basi ndazisiya, chifukwa chovala cha white kuchapira limodzi ndi cha Black sizimachita bwino nthawi zina. Now it is better I must be quite 4the moment, otherwise I can be in trouble 4 nothing.

 2. this are stupt things mot angosisa fees bat they wont people to get angrey OF ALL THE PRESDENT WHO HAVE been in malawi bat fees sinakwelepo chochi koma ziathuzinaz*STUPT#

 3. this are stupt things mot angosisa fees bat they wont people to get angrey OF ALL THE PRESDENT WHO HAVE been in malawi bat fees sinakwelepo chochi koma ziathuzinaz*STUPT#

 4. this are stupt things mot angosisa fees bat they wont people to get angrey OF ALL THE PRESDENT WHO HAVE been in malawi bat fees sinakwelepo chochi koma ziathuzinaz*STUPT#

 5. this are stupt things mot angosisa fees bat they wont people to get angrey OF ALL THE PRESDENT WHO HAVE been in malawi bat fees sinakwelepo chochi koma ziathuzinaz*STUPT#

 6. Shame, one story but full of Rubbish comments, Ophunzira samazitama padziko lapansi , achulukilenji ophunzira koma za chisoni kuvutika ngati sanaphunzire. Dziko LA Satan lodzadza n’ziwanda ndilosautsa Zedi ; zero point.

 7. Shame, one story but full of Rubbish comments, Ophunzira samazitama padziko lapansi , achulukilenji ophunzira koma za chisoni kuvutika ngati sanaphunzire. Dziko LA Satan lodzadza n’ziwanda ndilosautsa Zedi ; zero point.

 8. Nthawi zambiri m’mutu mukazaza uchitsiru, zochita zako, maganizo ako komanso n’zolemba zako zimakhala za uchitsiru ndipo pakamwa pazitsiru nthawi zonse pamatuluka zauchitsilu. Munthu wokhala ndi ubongo ogwira bwino ntchito sangamanyonze a police , pamene a police ntchito yawo INA ndi kuteteza pazipwilikiti ngati Mademo : I think many Malawian they are full of Rubbish in their minds, Oh ! Let me put it down .

 9. Nthawi zambiri m’mutu mukazaza uchitsiru, zochita zako, maganizo ako komanso n’zolemba zako zimakhala za uchitsiru ndipo pakamwa pazitsiru nthawi zonse pamatuluka zauchitsilu. Munthu wokhala ndi ubongo ogwira bwino ntchito sangamanyonze a police , pamene a police ntchito yawo INA ndi kuteteza pazipwilikiti ngati Mademo : I think many Malawian they are full of Rubbish in their minds, Oh ! Let me put it down .

 10. police shame to u,why u do brutal to our students nt thinking that ur kids one day they will be there now think abt ur wages shall u manage to pay xool frees

 11. Chimene anthu enainu mulemba simukuziwa chimene mukulemba kodi mavuto alimalawi anabwera bwanji boma tsilinalakwise kukwexa fees asafuna asiye chimene apolice anakachita anamba ana asukulu angapo kuti ena aphuzira atengepo phuzilo

 12. koma awadi ndi ana s xul anzanu akupanga nursing yomweyi paying alot of money osalandiranso kathu pakutha pa mwezi koma inu zambiri boma likukupatsani ulere koma apa muli busy kuononga zithu kodi 400000 inu mungadzalandire kangati sumx its not gud kumangopanga zithu cos kuti ena atero,,,,,,,think twice

 13. Indeed we are @ fees must fall campaighn there z no need 4 the police to assault prostesting students if u know hw it feels when u r coming 4m disadvantage famly!

 14. Kodi zafikanso pamenea? Ooo, koma kwavuta , koma bola mukanati muzitukwanizana nokhanokha Osantchulirana zamupanti mwa makolo, guys mukulakwitsatu ,nkhani yake itiyo pamenepa, Nooo ! Reduce your speed Guys .

 15. Galu + Fisi = Apolisi. Kalulu + Gwape = Ana odzindikira. Ntchito ya molalo koma yopanda malipiro ndiya Apolisi kaya sakuzimvera chisoni ndimalipirowo kuti azakwanitsa bwanji kulipira ana awo akasankhidwa kupita kumeneko. Department imene antchito ambiri amakonda kupempha kaya ndipamseu, muofesi kuposa wamisala ndiya apolisi. Department yoyamba yoti antchito amakhala mutumanyumba tonyasa ndiya Apolisi zachisoni panopa akulimbana ndi ana awo pa nkhani ya bwino ngati imeneyi n’kumati ndi ntchito yathu. Kodi mzakwanitsa inuyo kulipira nditimasalale twanuto? Bribes, kupemphapempha, molalo koma malipiro kuzanja ngati Apolice(MPS)

  1. Iwe Usalimbane Ndi Apolisi Kapolo Wa Dziko Pomwe Ulipo Uli Mbuu Ngati Thako La Galu. Nkhani Ili Apa Ikukhuzana Bwanji Ndi Salary Ya Polisi? Chitsiru Cha Munthu Iwe! Uneneso Uwone Ndikusaka Usaone Ngati Wabisala.Mbuli Ya Munthu Ukhale Ophunzira Ukanalemba Zanzeru Ngati Anzako

 16. Sorry for whatever has happened in school,that means those students need serious explaination from the schools higher authority

 17. Ajwinyeni nawo ma Jekeseni a poison aKAPOKOLAwo!! As if they are not going to be affected in one way or the other? Be civilised please!!!!

 18. So if u know the police’s duties, why don’t u go straight forward to them and tell them their own duties? Why don’t u stop the polices to put on Tear Gas? Masters degree ! Kkkkkkkk hahahaha, now why you are crying if u are more educated
  Bongololo sazola mafuta pagulu achimwene osamazita izi nzapadziko, do u get me ?

 19. ana opusa kwambiri m’malo moti azikaphumzira apa.chonsecho ana ambiri ndi amabwana amzanu akulira mu ma private colleges nde kumavuta ndi 400,000?

  1. #felix nawenso Pansana pako,#mathews musachuluke mzeru ndikukamba za chamba Simumandiziwa zomwe ndimapanga.#andrew sungadziwe kuti sindinapite ku unima or not cause inu ndine sitiziwana besides unima itha kukhala university yomwe mumaigomera koma sili mu top 100 ya Ma university muno mu africa.musadzionetse kuchenjera pa comment yanga tiyeni uko akapolo inu ozolowera zinthu za 2kwacha

 20. Akuti Ali mu high class , kkkkkkkk hahahaha, koma abale zomvesa chisoni, pomuwona ndimomwe alili ngakhale ma photo ake ndi high class very parallel, nchimodzimodzi mpunga kudyera thelere kkkkkkkk hahahaha . Stupid man.

 21. Manyeke apanyasaland akujaira guys, Kaye kununkha nkamwa poti kologeti is very expensive kkkkkkkk hahahaha, Mwana wapusi., chome .

 22. Iwe lonjezo chizunga, ngati ambwiyako anabwerapo kujoni kuno nkumavutika nde wamva ndialiyense ? Ubwere uwaone akazi anzako mmene akupangira makobili ,iwe ukhalira Uhule wakoomweo kumalawi kwakoko , Ukati ee umbuli ee umbuli Sukulu yake iti imene iwe unapia? Plz update inside of your underwear it’s smelling 2 bad, Futsek Hule.

 23. Man Samuel chipala, asiyeni ana aziwanda awa
  Akupwetekesani mutu . Sukumuwona nkhope anga chigoba cha nyawu kunchinji .Mwaiye chomwe amadziwa nkutukwana,mbuzi yamunthu.

 24. School fees is not the best way to collect money to run the Education system…..using technology Malawi government can collect enough money from general public and run all its ministries…Learn how to collect and protect the money.
  Make University Education affordable to everone.

 25. Wafika pontchula machende, eee koma uku nde nkuyaluka tsopano, mselu bwanji ulibe ? Ooo ndakuwona ndintchito yako kutukwana , kkkkkkkk hahahaha koma usamale udziwona nkhope pofuna kutukwana wamva iwe . Kodi ndiwe mwana wandani ukutukwana chotere? Ukuchokera mumtundu uti kumalawiko ? Sha ! Apa nde wafikapo.

 26. Koma NDE muubwira utsi uku nkuyamba, Usiru wachuluka mukufuna mukaphana muzati ee ee nthawi ya muthalika anthu amafa pomwe mukuyambisa dala nokha , muthalika plz can you send some more police man , akuzolowrra anthu amenewa kobasi.

 27. #UnimaFeesMustFall

  Am sure people now has come to their senses that Fees hike is indeed a general concern which need urgent action from the High Authority.

  Mbili zinzanga zimapanga blame Chanco, then Poly ndiye lero munena kuti chani?

  Sizoona kukweze fees mosaganizira chonchi. Kodi amene akukweza feeswo amakhala kuti? Ndiye kuti sakudziwa kuti Malawi ilibe ndalama and chuma sichikuyenda bwino?

  Anthuwa akuiwala kuti Revolution imayambika ndi Ana a Sukulu.

  COM go! Go! Go! Go! Until #UnimaFeesMustFall

 28. In five years time ,you will still have more hard Tear gas station, because of this stupid activities, why don’t u discuss with the Government nicely about school fees, then u’re busy doing nonsense, futsek. More fire Muthalika, show them your power ! They are full of Rubbish in their mind.

 29. boma la ana a maskin limeneli.zonse sizilibwino, njala ndimeneyi, zaumoyo sizilibwino,land bill ndimeneikuvutayi,education ndimene anyata akungthilidwa tia gas.KCN,POLYTECHIC and many more colleges and univesties,more fire ,,tiyenayeni peteryo. kuongola mtengo okhwima sikophweka zikavuta tingoudula.

 30. once a failure, and dats how he z, kaya sakuona kuti ma demo awa ndi sign wolephera kulamulira? mbavanso za a police zili yakaliyakali ndi ma teargas, ndiye chaninso

 31. Bwera kuno aise ulidziwe Dziko ,Osamangokhala pwiii malo amodzi ngati machimo achigololo kkkkkkkk hahahaha, ndiponso iwe ungolemba makomenti siiwe mwana wasukulu anta ndakudziwa ,mmesa umagulisa tomato mulilongwe munsika iwe nde ufuna kulimbana ndi wa jonzi , bladi fulu wako wamva iwe . Futsek zako.

 32. UNDEMOCRATIC PEOPLES’ PARTY (UPP) AND NOT DEMOCRATIC PEOPLES’ PARTY

 33. Tikanakondwa school ikanakhala yaulele kuyambila ku nkaka mpaka ku University, maiko ena ose salipila school ndi ku Malawi kokhakuno komwe timalipila

  1. Are you sure…. many countries pay tuition fees. The issue is with our economic struggles…Malawi yaonjeza, we just need the amount that is considerate with our income

  2. Sizimene anthuwa akufuna,, pajatu kwathu kuno timafuna zaulele nkuona kungoti mafuta akwela umva boma nkhaza,, school fees yakwela ayi president atule udindo pansi,, timafuna zaulele basi,,, Akufuna school fees yosika koma amafuna kudyako zankhuli daily

  3. Sizimene anthuwa akufuna,, pajatu kwathu kuno timafuna zaulele nkuona kungoti mafuta akwela umva boma nkhaza,, school fees yakwela ayi president atule udindo pansi,, timafuna zaulele basi,,, Akufuna school fees yosika koma amafuna kudyako zankhuli daily

 34. Ukudziwa chiyani mzanga chipala Samuel , kungoti njala ndiyoyomwe yaafola kwambiri mumajoint now that is why akungotukana President, akuiwala kuti iye akudyelera school yake . M’malo mopanga zoti iye ndi banja lake adye akungolibana ndi mfumu ,nde akufunananso kulimbana ndi wapajoni ,ndipo ndamusecha mafilo ake very poor.

 35. Kodi Nkhalambayi poti ili mu injury time basi ikuona ngati ikamafa dzikonso lizathela pompo. Go ahead fellors fight for a better tomorow

 36. Thank you very much man hahahaha, limenelo nde Dziko pamafunika ena osamba ena osasamba monga wanenara koma ngati alipo amene anakuuza kuti pajoni palibe mazi anakunamiza, just go ahead with what you are doing ,usalimbane ndi ine kuopera kuti zako zikawole ndikumanunkha, mind ur business, Futsek, u’re very Stupid man inja.

  1. Osamalimba ndi zitsiru ndipo or mutapanga review photo ake ndiye mupange anga mutha kusiyana bwana.thanks Evance mwawasegula maso

 37. Muthalika has failed us in Education and Justice in all his political career. As a minister of Education we had the same challenges and as a minister of Justice he introduced those undemocratic laws hence I am not surprised that we’re in these challenges once more, history is repeating it self here. He can be a good leader only if he can put in rightful people Ministerial positions not those greedy politicians like Kaliati, Chaponda, Mussa, Kalilani and Nankhumwa.

 38. I think this shows how stupid this Peter is. When will he address these university problems? Kumangodalira apolisi kuti athane ndi anao. Apolisi nanu kusowa nchito eti?

 39. Tiye nazoni until asinthe maganizo anthu amenewa,,,ngati amafuna kulemerela pa UNIMA akunama kwambiri

 40. Tazipangani ndi dzoko lanu losaukalo, simungadzimvereko chisoni ndizomwe mupangazo ,kapena mumangomva mademo.Malawi dziko la umbuli wazaoneni.

  1. Anthu akaphuzira bwino ndi kukhala Pachinto zabwino, azagula malata, cement ndikumanga nyumba kwa makolo ndi achibale awo,koma akalephera sukulu azabwelesa umphawi kwa makolo ndi achibale awo , dziko limatukuka ndi anthu ophuzira bwino

  2. they afraid of loosing their positions to gud educated and energetic people behind them,triple fees increase is a measure to limit us from being more than them….#Manchester 1-4#Borusha

  3. Nonsense how many of you chanco or poly graduates have contributed to the development of this sad country? its better to subside the locals coz the houses will stay in Malawi than some of you who live Malawi for greener pastures after benefiting from the poorest’s taxes.

  4. Nonsense how many of you chanco or poly graduates have contributed to the development of this sad country? its better to subside the locals coz the houses will stay in Malawi than some of you who live Malawi for greener pastures after benefiting from the poorest’s taxes.

 41. I thought police is busy with other jobs,(kingsley Dandaula watero kwa Billy Mayaya and friends against Land bill)…..why not keeping tear gas for The Tanzanians amene akutilanda nyanjawa..

  1. Ndiye Nkhondo Ndi TZ Yo AmamenyeRa Using Teargas!! ULIBE NZERU IWE! POLICE IS UNDEr home affairs and internal security! undifunse ndikuuze za ma duties of police mbuz ya munthu iwe!!

  2. Ken let me civic educate U on who am…Am well educated and a graduate with Masters degree..Siine Mbuzi as Ur..U cant teach me duties of a Police Officer..I know all these duties through Education not as a Stupid creature like U..Am warning U to take care of yo family yoself otherwise U will face consequences of your mouth…Watch your mouth brother Ken…Learn to respect people U dont know..I can pounce on U sooner or later..

  3. Can a constable threaten me on face book…Ur putting your job at risk brother…Watch your Mouth and concentrate on your job otherwise U will be noone on this earth..DPP is in govt U may be in trouble if fight against Me…Serious!!!!

 42. Dear Mr President. The police brutality against students is not a solution. But face, address and interveen the problem. Its not about party Mcp,Udf,Pp or Dpp but this is a serious problem facing our future leaders youth citizen. We cant have a mbuli future nation. Enough is enough, whatever the problem is its time u need to step in. Good luck students fight for yo rights.

 43. Musandikumbutse matsire apa chanco! Mupheko wa police mmodzi as a sacrifice, akujaira anthu amenewa! mxiiiiiiiiiiiiiii

  1. iwe pita ukaphe wapolice yo ngati ungakwanise,,y if u dnt hav anything to comment kungokhala chete,?kuzitenga wa nzeru ukuyankhula zopanda mutu,,

  2. Wauxilu iwe! nawexo ukumangoyankhula ngati wakhalira mutu bwanji? Ngati kuli wachibale wako muthoke akhale tcheru! mxiii

  3. The so called andy….then comment iweyo zanzeruzo other than criticizing other ppoz comments…u get no brains nigga…only if u had been at a university..SHUT THE FUCK UP..

  4. Vuto c opanga critciz comment bt uperi wamuvuta.if u/ur relatn z apolc man nde akafatu.. kd r u happy wth e fee hike?

 44. iiiiii kod a polisi vuto lanu ndichani?????? kkkkk apolisi bwanji??,,,….wishing you nice demonstrations,kukhumbira ndikanathamanga nawo those ma-demo!

  1. @ Andy hope u understand that the police is a goverment security department. Its not a political tool to disturb pple exercising their rights in a peaceful way. The police acts unprofesional even its a peaceful protest. Its time the police commision to tell the political leader that they are not the solution to the protests but the president is the solution to sit and talk with affected pple.

Comments are closed.