Rare comment: Police anger Gaba

police beat chanco students
Gaba angered by Police.
Gaba angered by Police.

South Africa based footballer Gabadinho Mhango has slammed the police for being cruel when dealing with Chancellor College students during the recent demonstrations at the college.

This is coming at a time when a video showing a police officer slapping two Chancellor College students has gone viral.

The Malawi international who plays for Golden Arrows posted the video on Instagram and captioned it with a message condemning police brutality.

He said: “Ndife amodzi. Mwana amafunika kumukonza mwachikondi osati nkhanza. Violence and brutality is a weakness but courage for negotiation and dialogue is maturity.”

Recently, human rights activist Rafiq Hajat who is also Executive Director of Institute of Policy for Interaction (IPI) slammed the police for their conduct saying time for police brutality is over.

“I think the days of police brutality are over and time to be accountability has come,” said Hajat.

He added that in United States of America police were caught on camera shooting black people and it’s not a good thing to see it in Malawi.

WATCH THE VIDEO BELOW: 

Advertisement

269 Comments

 1. those who rightly drunk ink r supposed 2 comment not including those nursery learner lk him . When students demonstrate freely they always damage other people’s properties in turn GVT pay 4 it so think twice b4 commenting please !

 2. Eazy….Makofi..sanalakwitse..watch out..Zomwe Apolice akuchita ku America…nde inu..khofi…mukalire bas….,,

 3. Enanu mungoti a police sanalakwitse it was a mare slap,were you the one who got slapped? whether a slap or beating,the law has to take cause,Police is not there to break the law,rather to in force it but not through physical torture.

 4. Don’t judge Gaba,he is a Malawian and free to comment on any issue concerning his country,enanu mudzafelamo not reaching level ya Gaba,with all your education.

 5. iyeyo gabayo anafikapo ku college…? chomwe angaziwe nd chot ana aku chanco akat avute sipakhala masewera…. only a slap ndye muzit nkhaza?nanga katundu awonongayo?

 6. School, school ya chani? Ku Malawi kuli sukulu? Litsiro lokhalokha langoti thooo ku Malawi. Kuli chani ku Malawi choti chingamatsangalatse wanthu? Si ku dzenje kutayirako dzinyalala? Mukumalimbana ndi zinthu za zii. Gaba walakwa chani? Kodi pa ma players amene akusewera mpira pa Malawi, kodi Gaba yekha ndiye mbuli?

 7. Once again, Gaba have proved to be a statesman. Thumbs up Gaba. It is people like you who can help this country develop. Enawa they just make noise pa internet, but in real life out there, they have no impact, their comments angothela pompa, your comments make impact, so does chanco’s voice. #UnimaFeesMustFall

 8. pple title police anger gaba nt education anger gaba,kuphunzira sikupita kuxol kokha kma kuyenda enafe kumayunivste tiliko kamba ka coruption evn kwanu chitukuko njema kma opanda nzeru pano akudya mam

 9. ndakumvesesa those who wanna compete with gabadinho nw they r late malawi wake ameneyu ngakhale ukhale ndi degree gaba analemera GOD gv separate thingz

 10. Gaba umbuli uli tho! akudziwa chani za police work. Mwenye uyu Hajat asamatero kufanizira za ku america ndi malawi. police works in the same manner you are performing. kugenda iyoyo kuthyapa. kupha nayonso slaughters; basi. “Do unto others the same way as they have done unto you”. mxiewwww

 11. Anawanso anaonjeza zoona angamanene kuti “Timkakuuza uzilimbikira sukulu usadzakhale londa lero ndizimenezi!”mukanakhala inu mukanatani?

 12. GABA has rite to express his vews over this,malawans look back uhad once ruled with not wel educated prezdent kma bwanj ulamuliro wake?unalitu supa,wat iz ineed iz humanity not those papers,apolisiwo must b ashamed of themselves,anangopezazerapo mwai ogwirako timadona ta xool powamenamo in the name of demo,iguess that oppotunity iz scarce to thiz gun men.

 13. Ndamva chisoni,inu amene timati munapita ku sukulu simungathe kumvetsa za ufulu wa munthu pa kulankhulapo zokhudza dziko lake.Shame.Mpake Malawi wosatukuka after 52 years of independence. Sizasukulu izi koma kukhudzidwa ndi mavuto adziko lako munthu.

 14. guys just’keep it up ,kaya!Analephera mayeso gaba inzo ndizake komabe!!!iwe ukudzintcha muphudzitsi uli ndi degree yako udziwerengera kut wapanga chan pamoyo wako !!!ndposo udzizifutsa kut Ameneyu gaba anayamba lit kuswera mpira ndpo wapanga chan !!!!osanena ngat smunapiteko Ku castle liga guyz

 15. The problem is the government ,they r using police to silence students which is not gud at all,but must remember what police did in muzuzu on 24 July,

 16. Ofcoz sukulu yo tilinayo, koma sitinganyoze Gaba, coz tikukanda now yet tilindi xul, and madzulo anoso tinapempha chakudya kwa aneba, pamene Gaba zake anachipila boom, though siwa xul bt alipenapake poti enafe tizamfa osafikapo with our education, ndipamene pangonela chinsisi cha Mulungu pamenepo, Mulungu anakati amapeleka luso coz of school enanu munakativuta2 apa, bt Mulungu si munthu, amapeleka kwa amane wamufuna!

 17. Munthu ukuti ulindi school and ukukandaxo hvy pa malawi panopa, nde ukanyoze Gaba coz of ma degree ogulawa agoti mbwee wa, Gaba anapita aixe, even iweyo ukuti wa sukulu we Gaba akhoza kukulemba job, and akupanga ma rands hvy moti ena a sukulu wo amamusilira atakhala mzawo, makape inu eti, Gaba ndi boss nw, wayendaxo hvy mayiko ambiri ndege yochita kulipililidwa ndi boma zoti enanu ndika xul kanuko sikazakufikisani pa Gaba, Mulungu si james mwamva, anakupasani xul yosapindula, Gaba anampaxa luso and akupindula!

 18. Mukulimbana ndi Bwana Gaba zake zinayera kalekale he is not even jelousy with anthu amene mukudzitcha ophunziranu thats why he has expressed his opnion ..enanu mudzaferamo ka Degree kanu kali mutapanga koma osafikabe pa level ya Gaba….shame on you nonse amene mukunyoza Gaba.

 19. They forget zat there a police when there in uniform once out of uniform there normal citizen wish
  @great cj gaba kumuona umbuli kwambili eti to be a leader its not xool or education they said to be educated doesn’t mean u will be rich or Mr knw it all BT minimise poolness

  1. Wapolisi amakhala wapolice, even when he iz in civilian wear he can perform his duties. uniform does not make a person to be a police officer but the appointment does simunswaone a cid inu kodi?amasiya kukhala a police chifukwa ali mu civilian wear?#UNIMAFEEMUSTFALL.

  2. @ Gondwa wht u should knw to be a police doesn’t grant he or she the powers to beat or harras any offenders which is the case of most of u pipo? Malawi police they life to behave a thug life you might not in uniform yet ur a police zat doesn’t make u a bull # FeeMust Fall

 20. ndimbuz zomwe kumunyoza gaba ali nd pepala la 4 ma D okhaokha azagwilisa ntchito kuchimbuz samakudziwan anthu olo size nd gaba c mungafane muzafa nd umphawi pozinamiza kut muna phunzira ana ambuz inu makutu ofana nd ujeni

 21. #arabson Muli Ndi Nzeru Heve,,big Up,,osati Mbuzi Zinazi Zikungokomenta Asakuzixata,,,,,,,kasalary Ka Wapolice Kangakwane Fz Ya Ku Unima? Nde Amandisekeranj Pakamwa Ndikumva Kupweteka?,,,,#fees Must Fall!!! Next Month Ndikubwereraxo Ku Xul,,woooooo!

 22. Mumapita mumakhara coordination do you think how he is manage if you people you call him mbuli zosaina saina amabwera mmanyumba mwanu kukuti mumu sainile ku SA komwe Ali amayankulako Chichewa pamoyo wake aw siku ndi siku muma muthandiza ndinu zofunakulemba kkk

 23. Tatiyeni tipite pa topic yathu nkhani ndi ya boma likukweza fees ku Univesity of Malawi and ophunzira anapanga chionesero posakondwa ndi nkhaniyi and a police pokakhazikisa ntendele anachitira nkhaza ophunzira Not Gaga’s Education Inu ophunziranu mukuti bwanji boma ndi a police.a kuchita bwino kutelo??? Fees ikakwezedwa tizakhala ndi mbuli zambili kumalawiko nfana ameneyu ndiwa nzeru okonda dziko lake kumenyana ndi boma ndi lulankhupo zikachitika chonchi then boma limabwenza maganizo kodi amene akusokoneza zithu mboma siophunzira mukuwafunawo akubanja ndalama siophunzira omwewu Kodi

 24. iwe ukunyoza gabawe khala chete ndika pepala kako kazigambako. police well done,dont entertain them.mbuli zaku chancozi tatopa nazo tisamango mvera iwowo.zili zonse ma demo ngati atopa kudya misonkho yathuyo abwere abadzalima mpiru kuno

 25. kupusa kwa amalawi ambiri sanachenjerebe amaona ngati xool ndiyonyadila mufufuze bwino bwino kuti kodi anthu omwe ndi ma mollioner ndiophunzira kapena ayi musamunyoze Gaba chifukwa cha xool kodi inu mkuphunzira kwanuko muli mchani???. kupusa simudaziwebe monsemuja kuti mu xool mulibe chuma koma munzeru ndimmene muli golde ndi silver???? siyani kunyoza osaphunzila

  1. anthu ambiri apa ndiosaphunzira koma amafuna azizionetsa ngati ophunzila… azizindikila patsogolo atalembedwa ntchito ndimunthu osaphunzilayo mapeto ake mkumazati wokhwima chifukwa chosavomereza

  2. Kwa ma comment onsewa ndiwe mmodxi wa anthu 5 alemba zanzeru,the rest dzitsiru kuyambira pamwambapo,Gaba is a public figure, he is talking sense

 26. Hihihihihihihihihihi mpaka gaba uja analephera jce pa mlauli walankhulapo???? aaaaaa basi izi ndi size ya gaba yomweyo ife tizakomenta za size yathu. Tingayambe kulowa nazo ku toilet yamafana olephera jce pa Mlauli. hehehehehehee

  1. Inuyo munakhonza JCE kayanso muli ndi MSCE koma titati tikufufuzeni mukhoza kupezekanso kuti mulibe kalikonse as compared with Gaba , musamanyoze amwene this is life sizingatheke kut wina aliyense aphunzire pa dziko lapansi lino, go and check education background ya the world Billionair Bill Gates then udzandifotokozere afta ua research ….

  2. Apa timati nyere yaponda njovu. A cj kodi m’mayesa ndi nakuvinilani tsopano mwayamba Ku shosha mavuzi,matendevu ndi njuchi muzikwanisa kuzigonjesa izi? bola mukana shosha ngumbi ndinakakuthandizilani Koma apa ine magweru sindikuwafuna.

  3. Gaba ali phe mnyumba yake yampanda magad ophuzla ali kunja akugadra iye, iwe even nyumba ulibe, palibe munthu amene aku kugadira usiku iwe ophuzirawe ukusowa yoblauzila kumene ukchita kutenga ngongole ndie ukuseka mzako iweo ndi amene uli mbuli pa malawi pano

  4. Hahahahaha fools. Stop this rubbish. who is that wingless insect after all. All those police officers were on their duty and did nothing wrong for this wingless insect to shout his noise.

  5. Vuto la malaw kukana chilungamo nanga gaba iye akudziwa chani za school we dnt care zoti ali ndi ndalama or not ndi mbuli basi sakuyenera akambe chiichonse chokhudza xul

  6. Kkkk Koma guys which is which apa?my eyes can only see 16th world war among us coz of this Gaba story let’s just live it,remember we all one.let sing”one love one heart let’s get together us one ena feel alright”.pliz brothers let’s just change the subject. l love u all. Thanks

  7. Mfana stev chalira, Ine sindinalembe jc coz ku geri kwathu kunalibe & ndiye tabwebwetatu kut ndinailemba kayani. I vowed not to be employed by an individual of my nationality wina iwe ukut maunits angongole chanchan tandipatse # yanko ndikubwezera ngongole ya pasavute ndi zachangu watengayo

 27. Nzika Izitelo Osamangoyang’anira Zinthu Zikuonongeka. Or Bankha Ukamafuna Kum’bera Mazra Amatekeseka Kusoza Umwini,what About Munthu? Onyoza Gaba Ndmbuli Kuposa Mbuli Zonse.

 28. Gaba raised his comment on the news that is curculating around the country just as like we are commenting here,but because he is a well known man you are commenting agaist him.nonsenu mukumunyoza iye sananyozeko munthu koma kunena maganizo ake kuzela mu comment ya pa news pa internet(print media)palibe mutolankhani wa malawi 24/42 amene wachezako ndi gaba pankhani imene alembayi nde because ndiotchuka azinyozedwa?, ngakhale inu amene msce certificate mulibe muli ndi itel wogwila facebook yokha mukulimbana ndi munthu woti zake zikuyenda you will remain poor.atolankhaniwa amapanga exagarate nkhani cholinga nyuziyo muikonde thus their business simukuona aika link apa you cant view it with free data.

 29. Uchitsirutu Umene Mukuchitawo Gaba Walakwa Chani? Mwasowa Zochita Asadzudzule Ngati Zalakwika Anthu Opusa nose mwakamba zaba enanuso ndi ku college komwe simunafikeko mwai ndi form 4 enanso mulibe koma kunyoza olomutakhala ophunzira kuposa gaba simunga fanane naye malipiro anu ndi ake mulikutalitali simungafikepo musiyeni nayeso amadziwa zoyipa ndi zabwino aaa! osasiya ayini akefe aku chanco tiyakhe bwanji? gaba akutithandizira enanu zisakukhudzeni mungokhala chete osati kunyoza iya vindele!

  1. mmmm! musavutike a chimwene nthawi ndilibe yomufuna gaba koma kunena chilungamo chomunyozera muthu ndi chani? amalawi sitingatukuke choncho mwaonjeza nsanje muleke

 30. Musiyeni Gaba kaya sanapite ka xuool bvuto lanu ndichani koma luso limene anapatsa chauta likupidulira akuposa munthu amene anapita ku xuool mwachitsanzo apolice enawa mungafanizire ndi Gaba

 31. Kkkkkkk,Gaba yemweyoo kuti wawawa.. Inu musalimbane ndi gaba,he’s earning alot wayenera kuyankhula,,2019 woo gaba MP basi..vote yanga nzakupasa

 32. Nkhani ili apa ndiyoti wapandidwa basi,kuchenjera mwaumbuli..mmalo moti azipanga zake iye nkumaanga ndemanga zakukoleji ngati akudziwako,ampanda pang’ono akanampatsa injury kuti apume ndimpira womwe kuti mwina angatseguke kumaso!

  1. Ndiye umbuli tikunenawo umenewo Gaba wapandidwa alemba pati??.Akuti Apolice amukwiisa Gaba.Mbuli u should go back to school idiot!!!!

 33. hahahaha maphunzilo pamalawi bola Gaba kudya money ,school yake ndi mpila ika khala fees ndizigoli zomwe amachinya. musiyeni Gaba

 34. Wapolisi sanalakwise guys. ….just a slap is nothing and more over ndili ku primary ndalandira mambama angati kuchoka kwa aziphudzisi? ?? They must grow. Well done Malawian police

  1. MALAWIANs we r too much soft that’s why amatiseka when we go out out of our country. ……I don’t mind even she can be my sister coz that’s part of her life training

  2. Nonse Ndinu Zitsiru Komaso Mbuli Simukudziwa Wat U R Talkin And How We Students Are Sufferin.Timalephera Kupereka 250 Ndye 400 Munthu Angaitenge Kut.Ngat Ndwe Mbuli Tseka Pakamwa Panu.

  3. The problem is not “Malawians being soft” its our literacy level that is letting us down. No wonder such ignorant comments. Those kids didnt do anything to deserve that kind of treatment.

  4. Ndinu mbuli ndichifukwa mukuchita support police. Mukaphunzira muzazindikira. Komanso udziwe kuti akumenyedwayo si anthu wamba ngati inuyo. Inu police kukumenyani nkhani ithera pompo hahahahahahahahaha

  5. I am not blaming your demonstrations Koma ndikudabwa kuti kambama komweko kumachita kukakomeza ngati mwina she was raped and killed lol lol wapolisi amadyadira tchito ???????

  6. i think zonsezi zikuchitika coz of poverty & ignorance,but ur demonstrations won’t solve anything,take t or not,think planib otherwise u r jst delaying urselves,inu zitchukani ndikuthyoledwa mapama anzanu tikudya kalongonda mwaufulu

 35. A changa wodya maye,musiyen Gaba.Iweyo nde mbuli theletu coz waiwala kut anthu ena analuza miyoyo yawo kut iweyo uziyankhula mwamtudzuwo.musiyen akuphanyila ufulu mazanamazana ya a malawi.zopusa,inuso apolic mundisamale basopo!!

 36. Tachokani apa ananyonyo inu Gaba zikumuvuta ndi mpila omwe angatiuze chaini apa zopusa basi ndichani amachiti chanzelu Gaba wanuyo mbuzi nonse ana onyela osatawasya ndi madzi

 37. Olo mumnyoze gaba,simungafanane nkhani ya dola,enanu ufa mulibe koma ndalama mwagula ma units onyozera gaba,mapwala anu,ndakwiya nanu

 38. i wish the whole country could join those students in those demos… misonkho yakwera kwmbiri… tikalipira misonkho anthu ake omwewonso akumabanso ndalama za boma

  1. omwe tili jozi tikulipilanso misonkho kwambiri makamaka tikamatumiza katundu tikumatchajidwa ndalama zambiri pakatundu wathu…. komanso tili ndi azibale.kumeneko akudalira ifeyo

 39. Copied…….

  WE MUST UNDERSTAND THAT GOVT DOESNT HAVE MONEY..WE MUST ALSO UNDERSTAND THAT UNIMA COUNCIL DOESNT HAVE MONEY THEREFORE WE MUST UNDERSTAND VERY WELL THAT OUR PARENTS TOO DO NOT HAVE MONEY TO PAY FOR SUCH EXORBITANT FEE @ UNIMA..!!! #FEESMUSTFALL @ ALL COST…!! IF GOVT DOESNT HAVE MONEY, WHERE WILL OUR PARENTS GET THE MONEY? WHERE WILL THEY PLUCK THE MONEY YU DEMANDING? ALL THOSE AT COUNCIL AS OFFICIALS AND ALL THESE saulosi CHILIMAs, mathews CHIKAONDAs, OKOMAATANI MALUNGAs,ralph KASAMBARAs, Maxon mbenderas, dingiswayo madises, 95% of unima lecturers were at unima, some frm very very poor families but govt gave them free varsity education, the kanyongolos , the annastanzia msosa, the charles tchuka and many many many more were at unima fo free, were provided with stationery allowance, free diet of chiwalo , beef and milk plus coffee, apples, pineapples, banana etc, free accommodation. Today they are educated, they are able to pay any fee for their children but do not want others to be educated as themselves. Th qstn is :wen in any country dd things become cheap? Things have neva been cheap at any point in tym but its about having good priorities and stop selfishness and greed. The hike of fee at unima means more salaries for those council staff, more salaries for lecturers, buying VX and 2016 model Fortuners, Mercs , maybe a Boughatti or Rolls Royce and othr benefits e.g holidays abroad, MASM VVIP class, free education for their children and we carry the burden to pay for that education, free electricity, free water, dstv subscription and other senseless benefits…the hike will never improve quality of education at all. We see these things in our colleges where lecturers compete in buying latest cars and building mansions. This NONSENSE of fee hike MUST STOP….we say #FEESMUSTFALLNOW

  1. dis comment z worth media en public attention osati zag gaba zanuzo zongofuna fame …..munthu wa za mpira chingamukhuze nchani kunkhani ya ma demo….

 40. Mukunyoza gaba why? Amalawi timalibana ndizithu za ziiii kuxiyaa zotithandiza enanu pa Gaba simugamake we go to xuool kuti tichose ubuli,iwe amene ukudalila xuool u die mene ulilimu educated savage ndakwiya nanu

 41. Mukunyoza gaba why? Amalawi timalibana ndizithu za ziiii kuxiyaa zotithandiza enanu pa Gaba simugamake we go to xuool kuti tichose ubuli,iwe amene ukudalila xuool u die mene ulilimu educated savage ndakwiya nanu

  1. Thus true big,palibe amapita ku xul ndicholinga choti azizangochulidwa kuti ndi graduate koma kuti tipeze ndilama basi nde ngati Gabayo ndilama akuipeza vuto alibe samaba.

 42. Funso langa kwa a Gaba inu za xool mukudziwapo chani,kodi inu mmesa idakukanikani atachita kukukonderani kukuchotsani mu STD 7 Kuti mukalembe a JC pa kalibu mwakagwanayo.

 43. Kodi abwampini inu Gaba walakwa chani kuti muzimunyoza apa??.Iye ngati mMalawi ali ndi ufulu oyikila ndemanga pa nkhani zanziko muno.Mukagwira phuno zanu nkumati eee ndi Gaba emwe,iwe ndiye ndani nyapapi ngati iwe idiot, fuck you all who are insulting dis guy kaks!!!:$:$:$:$:$

 44. ena pano mwangoti nyonyonyoo..nyonyonyo.! chonsecho mumaotcha kanyenya..zautsiru bax! musiyeni #Gaba alankhule..iweyo uli ndi nzeru koma anthu sakakuziwa..moreover mbuli yeniyeni ndiweyo bolaso Gaba. mwai facebook aah!

 45. malawi 24,2mol go 2 zomba central hosptal 2 c a policeman who has been serious wounded by chanco students & u can’t talk about a slap dat police gave 2 dat lady!Ndakwiya nanu a malaw 24!

 46. koma ngati nkhaniyi ili yowona apoli asiyiretu kuzunza anthu omwe akufuna kuzimenyera okha ufulu. Malawi asakhale ngati Zimbabwe. Ndikupempha a president ndi nduna zonse akhale pansi aganizire za anthu amphawi in the name of God

 47. Mmmh mpakana ndi a Gaba womwe? Mbuli ya munthu.Kodi kuchita ziwonetsero zikutanthawuza kuti muziwononga katundu waboma ndikusamvera wuphungu molingana ndi malamulo a dziko lino?

  1. amwene mmalawi muno tonse ndi ambuli..tikanakhala ozindikira bwezi malawi asali chonchi…droping out of school doesnt mean u are ignorant…to those ppo who have talents school is useless…here in malawi we think school is every thing…!!perhaps gabha can reason far better than you…#school is not only way of earning a living man…ghaba aanaka kuba misonkho ya anthu chifukwa cha timasalale tonyenyekati…

  2. Iweyo Ophunzira Ukuchitapo Chayani? Popeza Gabayo Nd M’malaw, Ndpo Osaphunzra Ndiweyo Coz Sumalikonda Dziko rako.

  3. Gaba ali ndi ufulu ngati wina aliyese koma ndikulakwa kumunyoza ndipo amene mukuti ndinu ophuziranu mulibe ndidzina lomwe,loti anthu angakambe.

  4. more over naye anangopangapo comment panyuzi ya nyasa times nde uzisuta kampopi nkumati agaba fwee!,sukuwona achita kulemba kut rare comment,foniyakoyo yovutanso network nkhumba

  5. #Steve school yake iti imene mudapita inu mpaka ku nyoza anzanu? Mbuli yayikulu ndinuyo man , munakakhala anzeru sibwezi mukuvutika choncho,, ndimakudziwani2 a Steve ….pa Gaba mudzaferamo osafikapooo…..think before you speak..kupusa

  6. Olo mutamunyoza Gaba, Gaba anavaya adha, iweyo ukuti wa school we Gaba akhoza kukulemba job and kumakudyexa 1 to 30, monday to sunday, and Gaba yo waponda mayiko oti inu a school nu muzafa musanafikeko, za Gaba zinayera panopa man, anthu a school wo akukanda hvy pa malawi pano, and amasiliraxo atakhala ngati Gaba!

  7. Asukuluwo akagwira kuti vep popeza azigogo awo anaphangira kale malo.let imkosi gaba alone ise wenecho tikumunyadira mwana wakwithu nangauli wandasambire kweni wanamakopala kulusa imwe mukukhumba kusambira yamaka.

  8. My question is which property was destroyed? I was there when all things were happening? Just hearing from any other media then you start commenting your rubbish that Chanco students destroyed the property. The police are the ones who initiated the violence and even burnt the hostel by firing a teargas canister which finally led to hostel catching fire. So what are you commenting Mr Educated intelligent unwise?

  9. Chitsiru Ameneyo Musiye Ali Ndi Certificate Ya Jce Zot Anthu Amakafika Ku College Samadziwako.Guyz Kale Munthu Wopita Ku College Amanjoya Coz Boma Limathandizapo Bt Nowdays Moyo Ukutilimbira Adasiya Kuthandiza But Kumakweza Fees Mwachimidz Choncho.Tiye Nazon Mbuz Zimenez.

  10. Reality is that the world does not respect the voice of an illiterate person no matter how wise he or she can try to prove to the public.He or she still remain illiterate whose voice does not hold any influence or authority on social,political and economic issues.An illiterate mind is a poor mind without voice and devoid of authority in society.

 48. Enawa alowesa chibwana pa bznes eti? Ngakhale ndi Ufulu wake ndiye Gaba eti? Mukufuna pochukirapo eti? This issue of fee hike is a sereous issue it need all off us to join hands against government not to jock with this issue

  1. Ndi Ufulu Wa Wina Aliyense Ngati ‘Gaba’ Kulankhulapo Maganizo Ake Pa Zinthu Zimene Zikukhuza Umunthu.Chomcho, Maganizo Ake Oti Apolisi Sadachite Bwino Kwa A Ku Chanco Akungoyenera Kulemekezedwa Osati Kumunyoza Just Because Ali Ndi Maphunziro Ochepa Ayi!

 49. what police did was absolutely good n this good cheap for nothing students think the gorvement is afraid of them kalua keep it up akwapulen akapitiliza

  1. what right s r u fighting for? rights of destroying gorvement properties n dont forget that even the wan who has never been at xul he or she z paying part of school fee n have u ever seen that person go on road n say i want part of my taxes to b used in reducing sugar price?????

  1. Koma amene anafela ufulu mukudyelawu si onse ophunzila. Pamene palakwika aliyese anene maganizo ake. Kuphunzila sikutanthauza kuti ndiwe ozindikila chilichonse. Mwaona apolisi odziwa ntchito bwino bwino koma kumaonetsa nkhaza pa anyamata a school. Gabayo anene zomwe wawona sikulakwa.

  1. et, mpaka “shit”? a Griffin mwaonjeza. mwalowa nkat hvy. mukanakhala inu mwanenedwa kt ‘shit’ bwa? dzkanakoma? si boh, amapanga choncho? mpaka apapa mmm

  2. guyz Gaba ndi angozo pano iye phee! kudya ndalama zake while inu mukunyoza. n sibho kulimbana ndimunthu odya zake coz alibe mulandu

Comments are closed.