Mphwiyo has last ‘Ralph’ as Bushiri fails to save his servant

Advertisement
Ralph Kasambara

The High Court in Lilongwe has found guilty former Malawi attorney general and justice minister Ralph Kasambara guilty of conspiring to murder the country’s former budget director Paul Mphwiyo.

Ralph Kasambara
Convict! Kasambara (in orange tie)

In a televised ruling, Judge Micheal Mtambo started by giving a background to the case and recollecting all the arguments that were presented before him.

In his ruling, the judge indicated that on the charge of attempted murder, he had found the two accused Pika Manondo and Macdonald Kumwembe guilty of the charge. In the second charge of conspiring to commit murder, the judge also found the two plus the former minister guilty.

Kasambara, a faithful servant of South Africa based self-acclaimed Prophet Shepherd Bushiri was once labelled by former President late Bingu wa Mutharika as a mafia.

Date for sentencing of the convict will be announced.

 

Advertisement

308 Comments

 1. Please leave Bushiri alone. Did Bushiri go to Kasambala or Kasambala went to Bushiri? This has nothing to do with Bushiri. Talk about other things.

 2. Don’t confuse, the are saying, they found them guilty of conspiring to murder Mphwiyo.. Its not Cashgate ndiye musati akafere kundende.

 3. Kasamba Anyongedwe Basi Wadya Mokwana Ndalama Zakuba Watilanga Ife wovutika Apolice Muvekeni Unyolo Kasambala

 4. Amalawi,amalawi amalawi tamvetsetsani bwino nkhaniyi.kodi bushili wataninso ndiamene anamutuma kasambala?mmmmm bodza bushili mumangodana naye moti mukapanda kumutchula bushili basi simuona bwino.mwina mmadwalatu sichoncho?

 5. Tiyeni tiwapase ulemu a Judge Ntambo for the well done job posayang;anira kuti uyu ndindani koma kuweruza mosakondela ndipo pomwe akuganizira chilango chake asazakondelenso koma achite chimodzimodzi zaka zoyenera mulandu wopha munthu. chifukwa chomwe chamangidwa pansi pano ngakhale kumwamba chamangidwa.

 6. Hahahaha malawians only tek luk on the negative xde wich aint Even true osakamba kut pitala a failin to feed his country bwanj every day Bushiri this Bushiri that mot ndalama akukulipilan yo azikagula chimanga kumakagaila anthu a mmudzi akusowawo ey are bizzy paying it 2 you anthu omvetsa chisoni mavuto onsewa inu bizzy bas pezan zina

 7. Haha I like the post end I like the comments …by de way hu is this guy u call prophet??

 8. Get the word ralph say that we overcome n whach n see n stop making misatake that ralph have west time on bushuri tiyeni tikubuke zomwe akanena kwa ndi pharist zinja dat wat z happebibg GOD of major 1 never fail

 9. Kunkhonde (mpoto) kwa Malawi, alongozgi wosi akulamuliya boma la Malawi, agone naku tulu cha pa ndale.
  Pe kanthu ko mwanandi ampupuka muziwa cha kutiyo Malawi wakwambiya pani?
  Malawi wakwambiya ku Nkhonde muboma la Rumphi ndi Rev. Levi Ziliro Mumba yo wangwambiska, Nyasaland African Congress, ndipu wangukolelana ndanyaki aku Nkhata-Bay ana Ching’oli, ana Manowa Chirwa, Kanyama Chiumia ndanyaki so aku Karonga ana Dunduzu chisiza brothers, aumali wenga ana Chibambo. Pa vuli ndikuzidana zina la chipani Malawi Congress Party mu 1959. Yo msanawale awusiyawo ana mulya weya wambewa.
  Asani mwewalawala pa wanthu wosi WO ndandalikapo, akufwa mwa chifukwa chimozachimoza ngemo wamangikiya yo Kasambara.
  Wenga Chakufwa Chihana mu1992, wanguzisinthaso vinthu muMalawi
  Asani mungawelenga lamsanawale unu mbalinga akunkhonde (Mpoto) Wo akufwiya za ndale?
  WO akuthawiya kubwalu?
  Woakusintha viwongu vau?
  WO akuthawa quarter system ya masambilu?
  Mumuoni nkhonde (mpoto) mowalili nge pa.
  Miseu yiwipe kumaiya pa Mzuzu/Mzimba M1 ndi M5 umaliya pa Muzuzu, WO utachifika Ku Rumphi ndi Karonga ngwa boma cha ngwa African integrated Road Cape to Cairo.
  Afwiyapu alinga amumaudindo nga boma?
  Amangikiyapu alinga kususkana ndalongozgiwo akandiya pasi Nkhonde (mpoto)?
  Ralph Kasambara ndumzuku Orton Chirwa Ku Lwazi, kweniko kungwambiyaso revolution, echekulutilizgaso mbwenu kumuwinga, awaanangwa, techenayu nkhondu ndanyiduwo eche kutikanda pamutu.
  Abayeng tosi cha mpaka so liwoondwi litundengi.
  Muoni museum wa M5 ndi M1 utalikiyana uli kutuliya kwa Jenda to Dwambazi? Chikangawa to Chintheche? Ndiso M1 wewija from Mzuzu Mall to Karonga?
  Wendi kanthu ndi Nkhonde alongozgiwo.
  Watuwengi Kasambara, ngwa pamphala, kweni wachenje ndi slow food/ clothe poisonings.
  Aaaaaaaaawe!!!!

 10. kusiyana pakati pa anthu osauka ndiolemera ena ntchito yao nkunyoza koma mau awo safikila onyozedwao pamene ena ntchito yao nkuzuza pomwe zowawazake zimakafikila ozuzidwayo

 11. guys we have to wait the sentence if the Kasambala get jail because lawyer is a crook something can change haah Malawi mostly are crooks even man of God is title of rich

 12. Nkhani apa siya bambo Bushiri,Yes…kma zoona xake ndi zot Ralph Kasambalayu anali jijiri jijiri kwa m’prophet yo kut mwina mlandu udzamuyendere ..Can I Prophesy to U Ralph Kasambala?…Bushiri kunfunsa Ralph…akasambala amvekere prophesy man of god/God ..hahahahaha “Ndkutha kuona Kasambala ali okhumudwa kut wataya nthawi,resources kuyesa ngat kut wina wake kunjako at kaya ndi ndan ndan angapangitse kut nkhan imuyendere.. hehedeee uluuh….Dalira Mulungu m’bale….watsoka otama mkono wanyama..Maulosi onse mmadzi kut chubwaaaa!!!! Zako izo

  1. If really Kasambara went to seek for solution at Bushiri it means he humbled himself. He could have chosen to go to sing’anga, but run to God. He is a God of second chance, no matter how hard the offence, God loves his children, cnd can show him mercy

 13. hello I’m Samuel Okizou by name, I’m giving a testimony about Dr.Sule the great Herbalist, he has the cure to all manner of diseases, he cured my HIV disease, though I went through different website I saw different testimonies about different herbalists, I was like: “Many people have the HIV cure why are people still suffering from it?” I thought of it, then I contact Dr.Sule via email, I didn’t believe him that much, I just wanted to give him a try, he replied my mail and Needed some Information about me, then I sent them to him, he prepared the CURE and sent it to me via UPS courier service, they told me that it will take 3-4 days before I’ll get the parcel, 3 days later I received the package and I started taking the medicine as prescribed by him, after 7 days of taking the medicine I went for check-up, I was tested HIV NEGATIVE… IF YOU ARE SERIOUS YOU WILL BE CURED!!! contact Dr Sule on whats-app +2348162447651.

 14. Children of God plz I berg u to hv love, Ambuye YESU Ada funsa funso akumphunzitsa omphunzira ake kuti ngati mu wakonda iwo okhawo akukukondani mungayembekezele kulandira mphoto yanji? Kondani Adani anu ndipo achitileni zabwino. Christu ananyozedwa,kulavulilidwa ndikumenyedwa bcz of Us ndipo Christu amalira nthawi zonse bcz of our everyday Sins but still amatikondabe. Tisamakondwele pamene anzanthu ali mumavuto tiyeni tiziwapempherera kuti amudziwe Mulungu. Chonde tiyeni tiyesese osamanyoza Anthu a Mulungu coz tikamatelo timazipalira moto tokha. I love u all Malawians.

 15. it has been a year now when everyday I am reading news on social media concerning Bushiri, its just Bushiri this Bushiri that, this has made me to realise that Bushiri is a great man.

 16. God have mercy on us….. Mayakhulidwe anthu afane nanu… Machitidwe anthu afane nane…. Help us ooh God to do what is right in ur eyes for we are ur children.

 17. am not for Bushiri,but this is not honest to say Bushiri has failed his servant, is rulph kasambara serving Bushiri or God?

 18. Ngati Yehova Mulungu wachiika kut nthawi ya moyo wako yatha, palibenso cholengedwa China chingathe kuonjezela nthawiyo

 19. I wish you people could read the article very carefully and understand it then comment…than most of these comments above. Anointed or not annointed, we are all children of God. Wheather or not Kasambara was laughing in court during the proceedings, the fact still remains that he has been found guilty and he is awaiting sentencing.

  No matter who you are or how educated you are…the long arm of law will one day find you and justice will be served. One by one you are going down slowly but surely. This is a big win for Malawi’s Judicial System….Keep it up..

  1. Lets not get involved in these issues. 1) Why Bushiri is involved on this story. 2) What connects Bushiri and Ralph. This case if u look properly, is a political orcherstrated. It is a political revenge. Thats why Ralph was laughing. Dont forget that if u are found guilty u have a right to appeal. So for them right now they are busy making a next move. Is the evidence strong enough to turn back appeal? He knows law, trust me he was just analysing their close arguments with Npa. U will be surpise with the appeal. They is no justice for political game. Justice is for those with money also. U and me we can talk. But they know the truth

 20. The founder of this page plus antchito ake ndi afit
  Chomuntchulila bushiri mkukhala chan
  Kod munthu olungama samwalila?
  Tiziti mulungu saona?
  & nkhani izi sizikugwilizana ndi ntumiki wanthu mwatintchulilai
  Plz repent guys

 21. Sometimes you think you are denting someone’s image by foolishly talking ill of him,yet you are indirectly making him famous

 22. Kkkkkk kalikwezeni dzina la #Papa wanthu #MajormajormajorAmenPapa,, osanda #Papa akutchukisani hvy2 ngati ndinu mukulamulira dziko, ngati sanatchure dzina lanu amamva kuyabwa2…..

 23. Note That There Also Suspended sentences where by any citizen of this nation is entintled to, you can also appeal against the conviction. Like General Kanene, You Can Be Pardoned.

 24. Amalawi tiye tivomeleze kuti bushiri ndi mutumiki Wa mulungu,anakulakwirani nchani?tiyeni tikapsele zenizeni osati kuyoza munthu Wa mulungu

 25. Ndinakuuzani a Malawi kuti andale akumalawi sangayendetse boma mwazionatu.Tatiyeni tiyese mbali zinazi mwina motowu ungazime.

 26. Now Ndakhulupilira Kut Ukakwera Pansana Panjobvu Usamat Kunja Kulibe Mame,mulingo Omwe Uyezera Anzakowo Mawe Uzayezedwera Omweo And Its True That The Hunter Will Become Hunted Kkkk Guys

 27. Koma ngati kuli zisiru zopanda dzeru ndiye ndinu, ngati wakutumani munthu wina mumuudze Kuti ndi chisiruso,,bushiri kondi iye anali ndi mulandu

 28. anakhara kut Ralph amatchula kut Help me God bwez atapulumuka koma pot amat PAPA Major 1 help me ndie ndizimeze2………Chipulumuso chili kwa Mulungu bac osat kwa Bushiri wasalano ukuwerengawe……….Babulo agwe bac!!!!

 29. Wasala ndi PITALA Namachende ameneyu tatopa naye, anapha chasowa komaso kuba mkati, Kasambala will be set free by the supreme court of apeal mungoti pheee muone.kkkkkkkkk. Ife tikufuna NAMACHENDE PITALA MBOLO YOSADULAYO

 30. Amalawi kusowa ponamizira eti akasambala inu mukutchula buchiri watani nthawiyake siino yotchulira atumiki amulungu mongataya nthawi pachabe mulungu anamsankha buchiri kukhala mutumiki wake ndare ,court,ndimauamulungu sizikugwirizana musiyeni buchiri aziweta nkhosa zake zomwe mulungu anampasa zaziii amalawi24 kusowa zolemba eti mulungu akukhulurukireni akumpando inu.

 31. Apa Ndiye Mulungu Wakumwamba Watiyankha Ndipo Afere Komweko. Ndalama Ndi Maphunziro Zalephela Kumupulumusa Coz Almighty God Alwayz There.

 32. Who is Bushiri?? Boma likhala likuonongabe ndalama apa………. Musayiwale kut KASAMBALA ndi okakamira. Imagine munthu oti akumvetsera chigamulo chake koma kumaseka ali mu khoti….

 33. Abale Mulungu samaimilila wolakwa kti awoloke ,Bushiri nchito yake siyoteteza olakwa nchifukwa ndimuneneli waMlungu ,ayiso alipo pakuolotsa wozuzikha nchifukwa Amene alimwaiye sanafune kuchitisa dzina lake manyazi musiyeni agwile ndikuolosa nkhosa zotaika ndikuzidalitsa osati kuimilila ochimwa

 34. Is about bushiri or kasambara hey!! poor mind writter malawi will never changed. Malawi nde kaya nzanuyu bushiri zake zili pa high kale is even known in all side of the world osamangodya mice yo bwa

 35. Ralph kasambara used to be a model in legal field but how can he commit such a crime yet he knew well the laws. Kwa iye wakudziwa kuchita nasachita Kuli ntchimo. So ndalama za u lawyer sizimamukwana up to the point of willing to kill somebody.

 36. Walakwachani bushiri mukuphatikiza zandale ZANU ndi zamulungu zikugwirizana soka kwa aneneri onyenga

  1. Mmmm Ayi Zikuonjeza Tsopano, Atakhala Kuti Kasambarayo Ndi Wa Church China Nkani Sikanapitirira Koma Poti Amapita Kwa A Prophet Nde Ikhale Nkhani? Bwanji Enawa Sanawalembe Komwe Amapemphera?

 37. Kodi ameneyu akusungidwa bwanji munthu WA mada?gryc tchinga painfa yake imamukhuza, kasambaraso; aaaaa gwileni basi nchigawenga. ameneyu osalimbana naye koma yapa ntanda naye,komanso osayiwala chaminga chipewa avale komanso azipulumuse yekha

 38. These 2 words Laugh and Ralph do not rhyme at all. This is a poor headline and just got to show how poor we are at using the queens language.

 39. zausilu basi kape bushiri alibe potetial mbalame yamunthu n ralph ku jere bas coz adalakwira laws ife sikuvaya geri coz of dem fuck em all

  1. man pachilichonse mungapange just know kuti zimakhala ndi zotsatira even utalapa komabe umalandila zotsatira. They is nothing bushiri akanapanga coz ndizotsatira zake.

 40. zina zili zose bushili?kodi bushili chakhala chitsononkho chotsulira zopusa zakuno kumalawi? zina zili zose bushili what 4? u guyz u must very stupid.take care with bushli

 41. My theory: Government will now turn to Mphwiyo in the cash gate case inorder to get at JB. Ralph will be used as a state witness in bargain to have his freedom back. JB in hot water. Watch the events as they unfold. I have spoken.

 42. Kusowa zolemba eti malo mumuyamikila muthu kuti wayamba kugawa chimanga chomwe Pitala akukanika ndikutiuza kuti tizidya mbewa ndi zitete basi iwe wagundika Bushiri yooooyoooo kusowa nkhani eti

  1. Nawe kuzolowera zolandira. Paja mu mipingomu mumapitilamo zolandira zomwezo. Gwirani ntchito muzigula chimanga inu. Zidya naoni za satanic zo

  2. nde ulesi amanena munthu uja umeneyo,kuzolowela kulandila zakudya kupingo malo molandila mawu aMulungu.nonse mukulandililatu mphoto yanu Mulungu sazakupasni yake mphoto.

 43. A Ralph apezekadi olakwa zoona? chouluka chimadzateradi eti ndie chilango chake sangomuutchelera bomba basi coz mfuti ukuchepera kkkkk boma ili likunditsangalatsa heavy pang’onopang’ono a that pysiti mkudzatsiridzira make gang’ayo

 44. Kapena Bushiri ndimulungu kapena anali mbon? ichi nd chipongwe kwa ntumiki wamulungu sizikumukhudza ndicholinga chake kupempherela anthu ovutika kut amasulidwe osat iyeyo kumasula ngat ambuye akhalachete ndan angayankhe, takumbukilan zija zidachitika nd prophet TB joshua anthu sitimamvetsa (meaning) ya prophet kod akakhala prophet mumpingo mwake anthu samafa? Amalawi umbuli ndi nsanje tizikhala chonch

  1. On.Tb josua….khan inali yoti….azipanga prophecy..paza anthu..omwe Anamwalira….ngat mowe amanenera za anthu ena…I remember even peter…sanane kut…anthu ake omutsatira sangafe ayi…koma Azinenanso….kut anthu anga ngozi ya imfa ikuchitikira……,,ameneuja nde opusaso kwambiri….

  2. Nkhan yonyozelana ndie iti kod mukamanyoza wena pa nkhan yokhuza chikhulupiliri ndie mumasonyeza chikhalidwe cha chi christu pepan (william)(gattusoh) ndilibe nanu chifukwa macheza apa enternet

 45. guyz anthu awa akuziwana kwinaku nkutitseka mmaso ,ngati zikumukhuza bas malamulo agwile ntchito ke ke ke zafika kwa aprophet eeeee

 46. Inu a malawi24 u r idiots link papa to this article. Kodi judas sanalangidwe atachimwa though he was a disciple? shame on you. leave papa alone. we know u write such artlz to attract more reactn poti more comments mean more revenue on your part. kudyera kulimbadi eeee.

 47. Mbuli zolowa mkalasi bambo.Timaganiza ndikuyembekezera kuti wina pokhala editor ndiye kuti ndiwozindikira.Bushiri zikumukhudza bwanji? Iye ali busy uko kupanga ndalama iwe uli busy kumayipitsa dzina lake.Ukhalira yomwe yomalipidwa ukawononga dzina la wina.Shame on you

 48. very stupid ndithu anthuwa anaba cash yambiri ovutika ndife misonkho yanthu yomwe apapa palibe za appeal akakhale ku jail basi ndende isamakhale kwaosauka galu ralph ndazake

 49. ,,,,,MALAWIANS WE ARE TOO BLIND TO FACTS,WE ALL ALWAYS MISS OUR OBJECTIVE AND FOCUS ON USELESS THINGS,IF KASAMBALA Z GUILTY AS CHARGED THEN THE QUESTION WE SHUD BE ASKING IS WHY DIS KASAMBALA WANTED TO KILL MPHWIYO,,,WHATS THE CONNECTION WITH CASHGATE,,OTHER WAYS THIS IA A USELESS PEACE OF SHT

  1. JUST BECAUSE YOU DONT LIKE MY COMMENT IT DOESN’T MEAN YOU GOT THE RIGHT TO CALL ME AN IDIOT,,THAT SHOWS WHO Z AN IDIOT BETWEEN THE TWO OF US

 50. Kodi anyani inu zumukhudza Bwanji Bushiri? Bushiri amagwira my high court? Bushiri wasanduka Mtambo? Or have they become brothers? Idiots!

  1. Happy how are u relating that in this issues……… Komatu penapake umbuliwu siwabwino don’t jux open ua mouth in useless tings

  2. hey!major 1 dint u knew ur servant’s court case,y mr bazuka doing this,where iz ur GOD during the judgement ,were he slept,bt worry not He has not yet done with u(kasambala)pray had,the master of major 1 wil c u thru.

  3. Mulungu wachina Kasambara nd Bushiri wagona…nanga servant wako akukalowatu Miracle pardoning bwanji…
   My Highcourt ndekut chani uhule eti

  4. pliz dont campare ur so called major 1 & JESUS safana olo nusu,za yesu zinalembedwa b4 he dies,so where they wrote kasambala wil attempt to kil mpwiyo & then arrest,who so ever followed JESUS & blived were helped,not just ur account wil b full of money,where from?u beta thinks u 2

  5. kma eeh! guyz let us nt judge that u may b judged also, mu nyumba ya mulungu muli mbale za ulemu nd zosakhala za ulemu, kaya inu muona kt bushiri nd satana ife sitiona choncho, w see God Jehovah. munena mpaka mutopa,

  6. Musamayankhule Choncho Ayi, Kodi Ophunzira A Yesu Atakanika Kuchotsa Ziwanda Kwa Munthu Uja Wamatenda Akugwa Ndiye Kuti Mulungu Wawo Anali Atagona? Musiyeni Mulungu Akhale Mulungu Palibe Chifukwa Chomanyozera A Prophet Apa, Moti Inuyo Simumapezana Ndi Mavuto? Ndiye Kuti Mulungu Wanu Amakhala Atagona? Abale Mulungu Simunthu Tiyeni Tizivomerez Nyengo Zina Zhkamachitika

  7. Zimamvetsa chisoni nkhani za bushirizi because anthu ambiri akutsatira za bodza amawauzazo muthatha kuona kuti kasambara ndimmodzi mwa anthu opusotsidwa ndi bushiri.

 51. Amalawi 24 ndinu mbuzi muzilemba zonveka bwino mukuchula anthu ambilimbili. Bingu analipo thawi imeney? Mukusowa zolemba mitu yanu ndithu

 52. Amalawi ambiri ndiwopengadi.no wonder peter ndi gulu lake akukudodani ngati mpira. Zagwilizana bwanji Bushiri ndi kupezeka ndi Mlandu kwa Kasambara?

  1. Basi Kudana Ndi Aprophet A Bushiriwo,ndiye Amangofuna Chilichonse Azipeza Ponyozera Basi,kusaganiza Mwanzeru Uku Chifukwa Palibe Zikugwirizana Apa!

  1. The one who comes from above is above all John 3v31, James 1v25 But the man who looks intently into the perfect law that gives freedom and continue to do this will be blessed. The law of the Spirit (thats the word of God is able to break the earthly law. With God all things are possible.

 53. Admin are u serious taking your time mixing stories which dont go along. However politically orcherstated cases are difficult to report. U are impressing yo superior. Bushiri, Kasambala, Bingu, and Authur they have lot of stories u can tell us one by one, without mixing

  1. william khala chete nawe Bushiri mmamukhumba eti tapangani zanu not za Bushir……wakhuta kalingonda eti…zaziiii muthu wamkulukulu kuganiza ngati mwana

 54. Paja ngati simutchula dzina la Bushiri mumachita zilubwelubwe, zikugwilizana bwanji ndi Bushiri? Kosowa nkhani komanso nsanje basi.

 55. Thank u God …..finally justice can b openly practiced in my land ….hop death penalty will start on diz gangz

 56. Thats why acountry it doesnt develop bcause of dis scenalio pipo ar busy consipiring instead of helping to solve counries problems

  1. Between you and them who are idiots ?You have no brain at all .The people you are saying are much far away richer than your poor Malawi .

 57. Really? Why does Bushiri’ name associated with this? Just asking
  ….! Can’t you do your work without mentioning Bushiri’s name?

 58. kikkkkkkk penapaketu ma admi muzakapsa moto ulele ndithu,bushiri walakwa chani apa?And ndikudikila chigamulocho ampase 30 yrs ameneyuhis time to reward.

 59. Mpwiyo is also going the same way since he was involved in stealing from us poor malawias so justice will have the last laugh not him…

  1. Why not just say Kasambala has been found guilty. How man clients does Ralph have. So many. Why choose Bushiri? It looks its a political orchastrated cases. That is Malawian politics.

  2. Atola nkhani opusa inu Stupid people zikukhuza bushiri zimenezi. Why do people die in an accident? Can we say God failed to save his servants ana a njoka inu.

Comments are closed.