‘Malawian men running away from priesthood’

Bishop Montfort Sitima

The Roman Catholic Church in the country has expressed concern over the shortage of priests saying the church is failing to serve the growing population in the country.

Leader of Catholic Church for Mangochi Diocese Bishop Montfort Sitima said the situation has come about because parents are not encouraging youths to become priests.

Speaking during Silver Jubilee celebrations of one the priests Medrick Chimbwanya, Sitima said parents have a role in contributing to evangelization by sending more boys for priestly formation.

Bishop Montfort Sitima
Bishop Montfort Sitima says the trend is worrisome.

“Today we are celebrating this Jubilee but in future we will not be celebrating because we haven’t been able to have new priests in our diocese,” said Sitima.

In his remarks, Chimbwanya urged Christians in the diocese to consider different vocations that are in the church adding that youths in the church should consider becoming nuns and priests.

“My friends whom I were ordained with when they were celebrating their jubilees they had some new priests being ordained but that is not the case here,” said Chimbwanya.

Mangochi diocese serves people in the districts of Mangochi, Balaka and parts of Machinga in the Ecclesiastical province of Blantyre in Malawi.

It was established as the Apostolic Prefecture of Fort Johnston from the Diocese of Zomba in 1969.

Advertisement

114 Comments

 1. Zanu izo nchifukwa chake akulu aja otchukawa nawo ayzindikila kuti this is rubbish ngati adam mulungu anampatsa nkazi inu ndinundani? Mmene akongololela tsikanawa wina nkumakhala gay for the res of his life thats madness at its best phindu ndi chani poti ansembewo ndamene akupeleka zimimba mmalocationimu za ziiiiiiiii basi

 2. Hello I’m Samuel Okizou by name, I’m giving a testimony about Dr.Sule the great Herbalist, he has the cure to all manner of diseases, he cured my HIV disease, though I went through different website I saw different testimonies about different herbalists, I was like: “Many people have the HIV cure why are people still suffering from it?” I thought of it, then I contact Dr.Sule via email, I didn’t believe him that much, I just wanted to give him a try, he replied my mail and Needed some Information about me, then I sent them to him, he prepared the CURE and sent it to me via UPS courier service, they told me that it will take 3-4 days before I’ll get the parcel, 3 days later I received the package and I started taking the medicine as prescribed by him, after 7 days of taking the medicine I went for check-up, I was tested HIV NEGATIVE… IF YOU ARE SERIOUS YOU WILL BE CURED!!! contact Dr Sule on whats-app +2348162447651

 3. Ku mlaliki akuti awiri aposa mmodzi chifukwa wina akagwa aona omudzutsa koma tsoka kwa iye ogona ekha akagwa asowa omtola ndiye iwe ukati uzigona wekha zachokera kuti Mulungu akhale opanda nzeru anzeru akhale iwowo za zii zeni zeni

 4. Iwe unabadwa ndima sperms abambo wako kupikisana ndi yesu mwanawa mulungu zotsatheka zimenezo chifukwa a bishop Anu a zuza ndimawapeza mu katawa akudikhula mzimayi pakana ana zausilu basi

 5. How can you encourage the youth not to have children of their own? I think this decision has to be personal at a certain age of their lives. Actually, something is wrong about this priesthood. Most of those guys have secret women and children and that’s double standard. By the way, you wouldn’t be there if your father decided to be one

 6. Osusana nafe athandizana nafe. Ife ndi akatolika basi. Ndipo mpingowu siuzafa. Ngakhale nonse osafunira zabwino mpingowu mutagwirisa nuclear weapons koma ife tizakhlapo. Proudly to be Catholic. Pakuti nkhondoyi akutimenyera ndi ambuye.
  Mwachidule mwini mundawu atipasa antchito okwanira. Ndipo ntchito igwiridwa

 7. kwa inu oyere mipingo Pliz konzani mitima nd makhalidwe kmanso zofooka xa church yanu nt busy with us…….. if u say we r dat n dat so wat, ? inu ndi olenga,? mesa ndinu olengedwa , ? kaya munene kaya mutani ife bola ndimulungu wanthu wamwambamwamba tukulumukizana #cathoric n proud

 8. Mpingo sukakamiza koma wekha umazimva malingana ndichiitanidwe chako. Ena adakwanitsa mpaka akalamba ali chomwecho. Zimangokhala mphamvu zasatana chifukwa okwatira atha kusiya nkazi wake ndikachita chigololo ndiwina tsono tisatengerepo mwai potukwana mpingo. Umo ndimomwe iye wasankhira.

 9. Chilipo chimene akuopa.sindinena koma ngati ukudandaula chonchi chimene chikufunika ndikukhala kuliona vutolo. Isaiah after noting that People are not getting him right he ” come now and let us reason together, says the Lord ” Isaiah 18:1 apanso chimodzi modzi mwina mutatero chifukwa anthu nde akufuna kufikirika ndi mau a Mulungu.

 10. Those are lies this church of Rome tells people. There are vocations, but the main problem is that the church is dealing with social status.

 11. Since religion is a scam based on lies and greed,what sensible person would want to enlist in that evil?
  Encouraging people to commit a crime can’t be legal,even for the Catholic Church.

 12. Anthu akuzindkira kuti ino sinthawi yolambira chilombo, asankha kupembeza Mulungu oona poona kuti nthawi yatha khrist alipafupi kwambiri. Tangoganizan #moyo_ndi_imfa inuyo mungasankhe chan? Anthu afika potopa nao uchimo mpaka kusalenda kut sakufunanso kuchimwira Mulungu ponama kut ndi a khrist koma akupembeza satana wachabechabe. KUDANDAULIRA; Tiyen tisunga Malamulo a MULUNGU ndi umbon wa Yesu khrist, tileke machimo athu onse, kupembeza chilombo, tikonzetsera mitima yathu kumulandira iye coz he’s very close than before. Amen

 13. Mumafuna mutafanana ndi yesu mwana wa maria,ndye mubamudikila naye pobwela kumwambako adzabwera ndi kanyenyezi koti kadzamuchose nkhawa zapamtanda zijatu.katolika umaganiza ngati mulungu ndi opanda nzeru eti ngati anachita kulamula kuti kwatilanani ndipo belekanani ngati mchenga wapanyanja so who are youuu?

 14. Cheating does not pay, for what will they benefit if they will put on the name of priesthood, koma ali mafumu azakudya?

 15. Kwa otsutsana ndi mipingo izo ndi zanu pakuti Mulungu sakaweluza chipembedzo koma ntchito zomwe umapanga ndi zomwe akaweluze iyeyo. Konda nzako ngati uzikondela iwe mwini.

 16. maitanidwe ndiosiyana,koma tikamalemba zolimbana ndimpingo tikulimbana ndimulungu mwini.ngati akhristu anthu ali ochepa tingolimbika kupemphera,akatolikanso adziwe kuti tsiku ndi tsiku akhristu akuchulukira ,chomwe chikufunika ndikulimbikira kupemphera komanso kuphunzitsa mabanja kuti aziphunzitsa ana ao zakulemekeza chiitanidwe

 17. june ndi july wamasikuano akusiyana ndiwakale , nde mutoti zoona inu munthu oti machine ake akugwira ntchito bobho uzikhala LONELY munyengo imeneyi. Isssaaah ma kiss atekinoloje ali yabviyabviwa uzingowayang’ana

 18. Ine ndinakanika nditasala ndi chaka chimodzi kuti ndimvekedwe usembewo koma ndinagolawa kutundu amene mukumudziwa ndi nangoti ( I can’t do this anymore)

 19. Munyongolo mmene umakomera muja nde usamamenye madzi asaaah,khala nawoni unsembe wanuwo.kkkkk ndikukalowa pentecostal churches.kkkkk eeeh abambo palibe amene safuna kugiligishana ndi nkadzi.kkkkk

 20. Tiyeni tipemphe mwini munda kuti alembe antchito ambiri. Mabanja aphunzitse ana awo kuopa Mulungu ndi kuwathandiza kusankha utumiki.

 21. Akatolika nanuso kuonjeza munthu angakhale bwanji osakwatiwa mumasatira Bible lake liti? Paul ati “kuli bwino nose mukanakhala ngati one koma chifukwa cha madama(zilakolako) mukhale naye mkazi mmodzi” ndiye inu mukuzitenga ngati oyeretsetsa pamene multi ndi zilakolako ndichifukwa chake asembe ambiri amachimwitsa azimayi mwachisitsi mpingo wachinyengo yezebeli!!!! Dragon power!!!!

 22. Ana amasiku ano akukonda kutosatosa,kulezela too bad sangakwanise atanganidwa ndizadziko awa.But u must know that dziko lapansi ndi Paradise kwa okanila malamulo a Mulungu and its Hell to those who worship God.Zimvele mumtolo.Proudly MUSLIM

  1. Not only that sanaitanidwe komanso vuto ndi ansembe ena amene amagwira ntchito mmalo osulira achinyamata omwe akuyenda mchiitanidwechi (seminaries). Ndaonapo angapo akuchotsedwa nkumati they don’t have such a vocation pamapeto pake nkukhala ansembe. So malo mowalimbikitsa amawakhumudwitsa

 23. Zikanakhala za Mulungu koma popeza mwangovala dzina ngati za Mulungu muli a Satanic mpaka kumasintha malamulo a Mulungu. Utha ngati katani mpingo umenewo

  1. Vuto lake ndilimeneri…busy kulimbana ndi mpingo wa anzanu,mavuto anu mwapsatira…chanzeru chomwe mungamachite nkukonza ubale wanu ndi mulungu…mipingo iyi ndingati zipani chabe,kumwamba kulibe izi

  2. Catholic church for evermore. Mwachepa ana ang’ono inu. Ngati yemwe anakhalapo wansembe ataukira analephera kuwugwesa mpingowu(Catholic) mapeto ache anspepesa kuti analakwisa kuukira Catholic. Nde anapempha Mulungu +Catholic church it self kuti akhululuke nde inu. Muli ndi soka

  3. Tsoka??? Go ask Benedict 16. Why did he resigned? Ndipo Kamuzu anali ochenjera anadziwa izi kalekale akanalimbikira zimene ankanena. Lero ndi izi zalowa mmagazi mukulephera kubvomera choona.

Comments are closed.