Am a mad person, says man who ransacked Bingu’s burial site

Bingu wa Mutharika mausoleum

He could not have any other excuse than claiming he is mad and did not know what he was doing when he broke into the mausoleum of Malawi’s ex-President Bingu wa Mutharika at Ndata Farm in Thyolo district where he destroyed several items before he was arrested.

If you ask one Ernest Mayaya Walesi for doing this he will only say he is mad.

Bingu wa Mutharika mausoleum
Bingu wa Mutharika mausoleum

He was arrested a day after the incident that has left many people wondering what his intentions were.

The 18 year-old was arrested on Monday for destroying six portraits of the late Mutharika, two serving bowls, two big drawers, window glasses, curtains, picture frames and other valuables.

While it remains sketchy on what Walesi and his yet to be known accomplices might have been looking for at the mausoleum, police have not yet come clear on the matter.

It is feared that the thugs might have had the intentions to sell the valuables. In the Mpumulo wa Bata Mausoleum Mutharika rests with his wife Ethel Mutharika.

Advertisement

143 Comments

 1. Ine zanga phee Kudikira Kuti ameneyu Apatsidwa Chilangochanji Akapezeka wolakwa? Nanga Chisiyana bwanji ndiamene Anagwidwa atafukula Mmanda Anthu achialubino?Kodi Satengedwa wakupha? Nanga achibale amalemu Bingu Ziwasangalatsa Kapena Adandaula Ngati Mmene amadandaulila achibale Aanthu Achialubino Manda awo akafukulidwa?

 2. azilonda akumandako anali kuti? mpakana kumulekelera munthu akasake ziwala mmanda akudziwana, komaso misala ndikumutu mumulange kuchokera pankhosi kutsika mmusimo

 3. He intends to raise the defense of insanity; a question of mens rea. It is one of the available defences in criminal law. Is such a defense available to him in this matter? Will it help to completely exonerate him? This defense has its own consequences eg detention at a mental health institution ( a social service for special groups).

 4. kodi ameneyu nesa amapanga mademo? simisala koma mademo ndiye alipo wa achitepo kanthu pazomwe akufuna ameneyo mapeto ake mpanda ndinyumba imene ija idzagumulidwa uyuyu akachedwetsa kuchitapo kanthu

 5. Leave that person alone
  Bingu is no more and he doesn’t know anything right now
  Don’t make people to suffer for useless things

  1. Akulu mutu wanu umagwira ntchito koma?utapeza munthu akuswa chiliza cha bambo ako unganene kuti musien my father z no more?

  2. my father was so much important to me he deserves respect, this man we talking here was master of cash gate, he left us in hot soup so I don’t care about him anymore

  3. You lomwe people are fools, you backing a person who stole a lot of money and build grave yard for himself left you on terrible poverty

 6. Komatu asalandire chilango choposa kukhala kundende masiku awiri,kapena kulipira chindapusa cha 12kwacha.aMalawi taona mmene milandu yaopha maalbino ikuweruzilidwa,munthu opha mzake zaka 7.

  1. yah i know where the killers are….. ndiwe mmodzi waiwo! so tell us were iz de mariketi?or ukakambila kusogolo

 7. Police apa nde mwapanga changu nanga bwanji za albino,issa njaunju sitinapange zachangu kungoononga tax payers money ife tikusowa panado mzipatala

  1. Aaah mudabwe coz ndi Za Bingu Ajah akufukula manda ama Albno Ajah mwayiwala kt nawoxo ndIanthu ofnika kuwapaxa ulemu

  2. Musayelekedwe agalu inu ngati pali anthu omvetsa chisoni ku joni mbava ndinuyo unyadile ndani akapolo ajons inu tchito kuitanila kaunjika wama nigeria shatapu

  3. Mmm,
   .abafazi akakhulumi kanjalo
   .akazi ambalonga tepo nkhabe tai
   .akadzi havatauri so
   .akazi sayankhula choncho
   .women do not speak like that

  4. kkkkkkkkk umbuli uli ndi ife aMalawi nde wamayi uyu kkkkk kuli xool kumalawi,umangomva xul nde ili pajinipo mwasiya ndikulandila zitupa za form two ukanene pali education.mukumvesa chisoni kusaganiza poyankhula.go n ask ur gvmnt abt the reason makes Malawi to b poor.first its poor educatn in Mw.bwela kuno uzaone xul n kwanuko tchito amafuna eprience kuno kaya ndimbuli ali nayo pachilichose.malawi first poor country in the world,who can b proud of malawi?kwaeni kuno kuyitanila kwaunjika ukunenayo rand yomwe amalandila paweek ndiya MP wanu kumalawiko.tazingopangani zanu papanjepo faz yapajon ikukongolesa malawiyo.ngati mulibe pata obwela kuno asiyeni omwe akudya marand.

  5. Umnamize ndani amene sadziwatu. R300 ndimene ukunyadila iweyo ndiwe opusa eti mp amalandila 12000 kwacha munangokula machende mulibe mzelu kuyenda mothawa apolisi mutavala silipasi pogona pamakatoni namanyonyo iwe ukhale chete mbuzi yamunthu olo unyoze malawi ndikwanube ufune usagune udzapita basi ukagonaso pansi pamtengo nanga olo yamaudzu uli nayo

  6. Lankhulani bwino chemwa, khalani ngati ndinu obeleka, mmene mutukwanila zikunditengela kutali kumaganizo. Ndi ntchito yanji yomwe mukugwila, abwana anu kapena ma customers anu amakondwela nanu?

  7. ndizowona komabe, ngati munthu wankulu simukadabwenza, ngati munthu akukutukwana pa gulu ngati ukubwezela owona amati nonse zitsilu, koma ngati udzichepetsa ndi kukhala chete ngakhale iye mwini amadziwa kuti ine nde chitsilu kwa zitsilu zonse

 8. Hahahahahaha sanalakwe nkulu anagona kumeneko anawononga zambiri zaife amalawi anzake nde mukadandaule ndizomwe waphwanya ameneyo, maka maka kumeko kukufunika bomba la petulo

 9. he is not mad anatumidwa bt it is so bad let us respect our let presidents soul Malawi this is inhuman, Malawi has change these days Malawi watani komaso ukupita kut kulimbana ndi manda, God bless my mother Malawi

 10. Tampatsani dengu akaike ku bafa ndikumuuza kuti akatsilemo madzi osamba muone ngati avomere, akavomera ndekuti ndiwamisaladi kamusiyeni ku mental ameneyo

 11. he should really be mad..how could he think Bingu was an albino?he’s looking for bones but hey,che Bingu kuyera kuja kunali kupya ndi kachasu….

  1. Ndimapanga check profile yanu mr jms mulewa, ndakupezani kuti ndinu a ku Ntcheu mwatuta kachewere nthawi yayitali.kenako munazapita pachichiri secondary pafupi ndi Chichiri Prisoni sory.Pano mukupezeka ku Salima pafupi ndi boma la Nkhotakota kuchimake kwa Chamba.Langizo langa kwa inu mr jms mulewa,chamba chakumeneko nchowawa gati simupezeka ku Zomba mukapezeka ku CHICHIRI Prison,kwanu kulibe chiriza cha omwalira kaya agogo anu??

Comments are closed.