I never said Zitete – Mutharika

463

President Peter Mutharika has denied media reports that he ordered Malawians to have grasshoppers for meals due to the hunger situation in the country.

Speaking last week, the Malawi leader urged citizens to be resourceful in their search for food and money, adding that they should not die from hunger when wild animals and insects were there for them to eat.

Peter Mutharika

Mutharika: Changes tune.

However speaking during roads inspection in Zomba, Mutharika said he never mentioned Zitete but rather “Zicheche” which is commonly known to be yams in his district of Thyolo.

“I never said Zitete, I said Zicheche, Zicheche in my area can be referred to as Yams not the grasshoppers. People always misquote me, this nonsense must stop,” said Mutharika.

But he was quick to say that rats locally known as “Mbewa” are delicious hence Malawians can have them for meals due to hunger. “Mbewa is delicious, I even had some for my dinner last night,” added Mutharika.

Earlier, Social commentator Felix Unyolo faulted the president’s remark arguing that the hunger crisis in the country should not be regarded as a mere joke.

Share.

463 Comments

 1. Amene sanachimwepo atole mwala agende nzake kodi inu pamoyo wanu mumachita zolondola zokhazokha simulakwisa?chonde yesesan musamachite kudzionesera kut ndinu mbuli,,,,, muzingosaukabe iyeyo akusangalala nonsense.

 2. Coment loadin or ndi komente ndikhala chimodxmodxi ngt ndikusowa chakudya sikt ndikanyoxa kapena kuwayamikila amutharika ndixipexa ai, iwe ndalama kwaiwo sinkhni, ma president onxe akhala akubwerawa palibe chimasintha paine ndi mmene ndilili iwo akungoxinenepela, apresident iwo alibe problem xawo zili smart so ine mvutikile chani ndimaphuxo mmalo moti ndipange xanga iwo makobili ali phwi kuchta kusowa poponda kunyumba kwawo zaziiiiiii

 3. A horn Peter waMuthalika watelo nanga aNkasa alikuti ayimbenso.Jodi siaja anayimba za mikhaka zimene ananena aBakili?Peter IRA indeed uneducated idiot.We thought is smart ,Let’s see he will go exile like his late brother and sister Joice.This is Kamuzu’s Malawi tikakwiya sitipanganika.

 4. Munthu amanyozedwa kmanso kulemekezedwa chifukwa chakhalidwe lake sibwino kulemedza munthu oti salabadira za wina sibwinso kunyoza munthu amene amaganizira za mavuto awina

 5. Vuto kumalawikuno ndi a midia malo motumikira ntunduwamalawi inu mulibzy agnest president munavabwinobwino kuti zitete kapena kut mpama bt inu mwalowesapo ndale penapake inu ATORANKHANI tazikhalani feya pantchitoyanu ndiye mukuonangati nsogoleri wa 100% muzamupezakut? Wina aliyense alindizofooka zake oro aliiweyo madala ako oro amako tiwapezelanso zofooka Tiyeni ife amalawi tigogwirana manja kuti zikolanthu litukuku bas

 6. Isn’t it interesting that the same person who was busy correcting parliamentarians’ language problems a few days ago is complaining of being “misquoted” due to his failure to articulate chichewa words well? Mr President, what people need are straight forward solutions to their real problems. if its about crop diversification, that can be implemented and is a continuous song that people already know. but people need salvation from today’s hunger before they can start planting “zitchetche” tomorrow.

 7. Malawi needs a dictator President , we should not blame only the President start with ur mp and minister what r they doing in the parliament and if ur a Christian knee down and pray to God that next we should have enough rainfall

 8. Malawi needs a dictator President , we should not blame only the President start with ur mp and minister what r they doing in the parliament and if ur a Christian knee down and pray to God that next we should have enough rainfall

 9. Ndingayamikire bwanji mtsogoreri emwe even m’dziko muno chakudya chenichenichi ndi vuto la chaka ndi chaka pomwe maiko azathu akamati kuli mavuto ndie kuti akusowa ma tv, magetsi ndi zina zoti olo atapanda kukhala nazo moyo umaendabe sikuno msima ndi golide masiku ano olo ya therere. Ndie mkumati dziko likuenda bwino NO SENSE

 10. Ndingayamikire bwanji mtsogoreri emwe even m’dziko muno chakudya chenichenichi ndi vuto la chaka ndi chaka pomwe maiko azathu akamati kuli mavuto ndie kuti akusowa ma tv, magetsi ndi zina zoti olo atapanda kukhala nazo moyo umaendabe sikuno msima ndi golide masiku ano olo ya therere. Ndie mkumati dziko likuenda bwino NO SENSE

 11. That’s why kumalawi achinyamata akuthawila maiko ayiniake coz they loose hope kuti tsiku lina zinthu zizasintha,amalawi si awulesi try to create jobs for us,tel the chinise kuti ngiti akufuna kupanga bizness azitsekula ma company ndikuwasiila mashop eni dziko

 12. Atsogoleri amalawi ndi adyela ndi kuba,amawona zawo zokha,for example nkhani ya Njala boma likupangapo chani,kodi kumalawi kulibe malo oti boma likhonza kusegula ma farm kumpoto,pakati ndi Ku mmwela ndikumagwilisa ntchito akayidi?,Malawi ndi dziko la mtendele koma atsogeleri samawakonda anthu awo coz they r after money nthawi yawo is an a the.

 13. Kodi2 olo kutakhala President otani kunyoza sikungathe amalawi timangodziwa kunyoza ndi sanje mpake chifukwa dziko lathu silizatukuka chifukwa ndife mbuzi

 14. Poor journalists. Shame to you. Sometimes its not good to be the first to write and air things. Shame. Correct yourself . What do you have to say then.

 15. Mugabe two uyu hahahahaha zinango fika ndiku nkanika zinthuzi basi ndizo enela akulu akulu omwe aja aish izindezina chiku ipitsa mbili ya #DPP ichi anla

 16. Guyz zina lina la ZICHECHE ndi MPAMA in English Yam ndiye inu ngati simukudziwa mudziwe lero a bwana sadalakwise musiyeni proffesor AZIUFILA ndi bambo athu BASI.

 17. KOMA PRESIDENT WATHUYU NDIYE NDI MABVUTO KWAMBIRI, CHIKHALA KUTI AMAVOMELA KU EXCHANGE, TINAKA CHANGE ,SOMETIMES KUPHUNZILA KWAMBIRI NDI VUTOSO ,MUNTHU UMADZELE DZEKA, MOTI PANOPA PRESIDENT ATHUWA ADZELEDZEKA BASI

 18. Kodi amalawi mpaka liti muzakhale mukulalatila president wanu?MULUNGU amati muzipempherera atsogoleri anu no matter what,so you can’t change on this,you will keep on suffering.Mvula ikavuta bwanji simulalatila president,why counting other people language leave your? .GOD,FORGIVE MALAWI.

 19. Kodi amalawi mpaka liti muzakhale mukulalatila president wanu?MULUNGU amati muzipempherera atsogoleri anu no matter what,so you can’t change on this,you will keep on suffering.Mvula ikavuta bwanji simulalatila president,why counting other people language leave your? .GOD,FORGIVE MALAWI.

 20. Pepani sitinakumveni bwino koma vuto ndiloti chichewa chimakuvutani koma Mayi Kaliati anamvani bwino lomwe chifukwa iwo anati mumapanga ma jokes, ngati nokha nokha sikumvana nanga ife tikumvani?Akuluwa akunama kuteroko ndi damage control akuchitayo.

 21. abwana musakane lero poti mwayaluka.atolankhani.sakunamizila.ma records anu.tilinawo ndie tionesapo pa TV.malawi.tione ngati sidzowana za grasshopper mun’kayankhulazo.amzanu.achina muluzi.amapanga nthabwala koma zimaoneka kuti izi ndinthabwala.tsono inu munayamba ndinkhani.ya grasshopper kusonyeza kuti.man festal anu.ali Ameneo ansonkhano wanu?

 22. Nkhalamba zandale zikuvutisa ma born free! ! Now days…kenako tinva malawi country iz on for sale…!! Iwowo nkumapita kumudxi kwao..
  ..amene mmunkawanidza ndi omwe …!! F**ck ..mabo.bo..n stop blubling us wr pple..timanyera manyi ofana even tidye mbewa zitete wit deya ..wat so ever mmimba simukana bola manyi..again long finger on you! !!!!!!! Y

 23. Malawi is full of critics than innovators. We need to change and help the President build this nation, or we will be poor forever. Chitukuko ndi ufulu zomwe tikudziwa ife ndikudzudzula basi. Worrisome!

 24. Mr president , please do good to your people and apologise us rather than arrogance. There are only 3 years to go, we are watching you and hope we will never vote you again. It is written in the BIBLE “Pride is before a Crash” by king solomon….

 25. So the president and Kaliati now seems to differ on the same, Kaliati said the president was just joking here pitala is saying I did not say zitete I said Zicheche, who is fooling malawians here, mind you Mr president, that evrything you said is recorded, should we play back what you said?

 26. Vuto lamalawi mumalimbana ndi zinthu zopanda pake aliyense amalakwisa musanyoze ntsogoleri wanu ingomvesetsani kut analakwisa bas, mwaiwala zabwino zomwe wachita koma kunyoza bas

 27. president is one,not one & half or 2.In the time of joyce,bingu,bakili,there was hunger,people were killed,things were very expensive same as this days.no leader will 100%,its only God

 28. These pple cannot even put their heads together, they are busy contradicting each other without noticing. Today the president say pple must eat zitete and mbewa, tomorow the minister of information comes with her damage control saying the president was joking. The following day the president comes again and say, i said zicheche not zitete. Kodi boma limeneli bwanji phada wake wa ntundu wanji. Reasoning ikumaavuta pati.

 29. That’s is your problem amalawi inu you don’t know nothing but chimunthu tchankhaza munachivotela kale kodi munthu manyi wanya yeka angadyeso munamuvotela nokha lelo mukumulila ine nakwaine vuto ndinu anthu bingu is his brother you don’t remember what he wants doing kodi kungochipitsa manyuwa mwati anthuwa ndi abwino but just say Amen mulungu pali chimene angakhoze

 30. Pliz,we r tired with lies,hunger,drug shortages,high taxes,to make matters more stink failin to pay civil servants in time,beta zimbambw tu apa!!

 31. Man panopa yalakwa palibenso canzeru chimene ndikachinve kuchokera kwa inu man anzanu onse amayesako koma inu man eeeh mwatikwana heavy mungopakiliratu man mwachita exipire ukongwaa

 32. akutsutsana okhaokha ndi minister wake wa information,a kaliati atiuza kuti munati zitete koma ma jokes,inu mukuti zicheche,timve ziti

 33. Why silent all this time and fooling who? Yu are not the only one from yur area, why they didnt come open defending yu that yu were reffering to yams. First stop yur nosense then we will stop our’s. Remember, yu are a head of state, looking after Malawians, regardless of tribe. Yu mean there was no interprenter and yur speech came accidentally.

 34. Mr president fulfil ur promises u made during campaign one of them is to eradicate hunger, so stop making nonses jokes to the pipo who voted 4 u or else resign and go where u belong. We are tired of nonses

 35. It was same issue with Kamuzu…Muluzi..Muntharika Bingu…Joyce now its Peter….whatever you do good or bad people always find something negative to say..so keep on critising presidents muzazindikira mwakalamba muli amphawi choncho…kukhala president its not easy thing and dont forget kuti tilibe ma resouce obwelesa ndalama kwathuko thats y country is poor..but mutafuna only u people can be rich ngati mutakhala anthu olimbikira than wasting ur time talking much about presidents..

 36. Most of times I strive to steer away from controversies of Malawi Politics. But I can’t help it. Now that APM has clarified on the mistake on Zitete/Zicheche, now what happens to the statement issued by Hon. Information Ministry backing the President’s Zitete joke? Are they required to write a fresh one or withdraw the statement and pretend they never issued one at all…#justthinking

 37. Anapagali sinanga mumadya zitete ndiye chavuta ndixhani apa ndimaganiza kuti mwina walakwisa wati bwewa ndi manyi or zitete ndi manyi koma inu zinthuzo mumadya kale agalu inu ndipikisana nanu

 38. #BWAAAAAAAMPIIIIIIIIIIIINI opanda mano..as a president how can you tell your pipo kuti azidya zitete & mbewa then pambuyo nkumakana kuti you never said that,are you MAD mr president peter BWAMPINI mutharika?

 39. Slung slang poyankhula abwana .speak like aniggar you have been in US .long time you still speak like you you just arrived from Congo your original ancestors land.

 40. Mr president, people knowingly choose to misquote you because they know that is the only way they get attention because when it comes to development, vision for this country and your love for the people, they can’t come close. Don’t mind them, Ntchito ZANU zikukuchitirani umboni, a president. God bless you

 41. OK point ya zipwete tamva wapanga correction,what about point yambewa ija unama kuti chaaa? Pitala ua shupiti may u stop say lies to my nation over wise go to hell
  You can’t joke nkhani yanjala with pipo empty stomach

 42. Ku SA kuno nkhani imeneyi ndiye tikusowa nayo mtendele osati masewera aliyense angotinena kuti tinathawa kudya zitete ndi mbewa kwathu, ndipo ndiye tayaluka tikingokhara ngati zitsilu, chilekwa cha president ngati ichi sinachioneposo ndipo zamanyazi kwabasi

 43. This contradicts wateva the minister of information told the nation, this shows that he regrets it now, n now r those zicheche available at Admarc n mbewa? No visionary pple in driving seat!

 44. Kkkkkkkkkk mr president, do you think that people they don’t understand what you said? B4 you say something you must think. Don’t say nosense and tomorrow change yuor mind.

 45. thank you for clearing up this Misunderstanding Mr President! kwathu mbewu ya Mpama/zitchetche/yams inasowa koma utapezeka mwaiwo nkutigulitsako ndi chakudya chabwino! Zikomo

  • Most of times I strive to steer away from controversies of Malawi Politics. But I can’t help it. Now that APM has clarified on the mistake on Zitete/Zicheche, now what happens to the statement issued by Hon. Information Ministry backing the President’s Zitete joke? Are they required to write a fresh one or withdraw the statement and pretend they never issued one at all…#justthinking

 46. Mr president sir why u ddnt say,,,, kumadyanso #BWAMPINI,,,,,,,,to those who eat that thing akanadyako chibwampini chichikulu,,,,,kķķkkkkkkkkkk

 47. malawi amakonda munthu akapita…..mumakhala phee mwakwanu osamalima mumandikira president…ndivute lake kut nvula sinegwe mukwanira?…..think some tym….musanayakhule……iyaaaa

 48. He needs mouth & tongue operation…sadly,surgeons are told to venture into entrepreneurship…no job in Health sector under Malawi Govt…Misspeech tatamounts misqoute,u’ll bear with us Mr President..

 49. malo moti mungwile tchito zanu mukufuna pita akupasen chakudya osangwila tchito asadye ndindani muzamuyamikile pot onse mukuti oipa ndiye kakhaleni inu ku stat house

 50. Shame!!!!!!!! Kwa one anavotela mbuzi ngati imeneyi yoziganizila yokha anthu ena nkumawatenga ngati zitsilu munthu opanda uzimu osapemphela ngati uyu udyeletu sudzawinanso mizimu ya Malawi singamakhale ikudandaula iweyo Mulungu akukuona ndi poor glamour ngati chichewa sumatha osangosiya kuwa panga anthu address bwanji uzingodya za nyovwinyovwi kwanuko bwanji munthu opanfa chisoni unachokela kuti tatopa nawe ife.Mulungu Ali mbali yathu you’ll die like a dog.

 51. Kodi bwakukakamila kukana zinthu zomwe aMalawi anakumvani mukunena ndipakamwa panu bwanji ngati munanena kuti zicheche ndiye chinalakwika ndichani kuti Kaliat azizati the president was joking what so funny about kutchula dzina la zicheche in ur area,komansotu munatchula kuti aMalawi azidyanso mbewa ndiye dzina limeneli mulitembenuza motani mmatchulidwe ndimmatanthauzilidwe a kumudzi kwau coz pa zitetepa apa watibwatika kuti sizitete koma zicheche ndiye tikudikira mutiuzeno pambewapa kuti ndichanino

 52. anthu ena mukumalemba makonti atali ngati nkhani koma opanda nzelu,munthu walankhula zopusa nde wina nkumati anthu mumayang’ana zofooka zapulezidenti!zopusa anthu akuvutika muno,kugona ndinjala.

 53. Why did we vote for someone who has never grown up in Malawi? who doesn’t know how to speak properly one of our Malawian languages?look now,our President is embarrassing who makes mistake one after another

 54. Amalawi tonse tomwe tikunyoxa president ngati muli akadzi nyini za manjazo mahule inu amuna nonse mwanyoxa peter mbolo za panjazo anyani,ana amasiye,ana afiti machende siyani kuyakhula zopusa tingoonesana 2019 pama vote ndma president anu opusa amalawi zitsiru anthu okuba dziko la zitsiru kmaso anthu okuba opanda nzeru malo momuthandiza president kuthesa khalidwe lopha azathu achi albino kma busy kukamba zopusa khan zoti zachitika zatha kma bsi kukamba khan mpaka chaka pamene abale athu achi albino akuphedwa ngat khuku ndi anthu omwenu omwe mukuyakhura zopusanu muthu wanjala angapeze mphamvu zophera zake malawi mulibe njala akula ndimaluzi thats y GOD IS PUNISHIN US WITH HUNGER COZ WE ARE KILLIN EACH OTHER MUDZINA LA UPHAWI,MALUZI KMASO NJALA

 55. The president must admit that he made a mistake by joking in nt ryt time. even atakhala kuti ananena Zicheche was t ryt to say that? nanga mau oti makoswe analakwisanso sanalankhule?

 56. OK, whether Combusus or Columbus provided u get the idea. Zikafanana matchulidwe chilichonse chimakhala cholondola akakupanikiza. ” I did not say that or this ” comes at the end koma imakhala regret after making a mistake. Sorry Mr President.

 57. I regret being Malawian. Wen wl our country achieve its goals. Every year it’s all about hunger, ee this & that heyiiiii

 58. apa bwana ingovomeleza ndpo za zitete evn pa kanema yatha anaonesa ztetezo,, ngumbi nd zna zotero bwanj smufuna kuvomeleza zolakwika koma kufuna kulimbana nd amalawi amene ali pa ululu wa maluzi??

 59. stupid journalist who always misinterprete somebody speach inoder to make him guilty btwn the crowd.

 60. I support MCP koma nkhani iyi ndiyopanda ntchito please atolankhani taisiyani siipindula. Leave the president alone and dont disturb his work. This isnt fun and tatopa nazo ife…MCP 2019 BOMA!!!!

 61. Anthu anamva zomwe mudanena achakulungwa.alomwe ndi alomwe anamva zimenezi.akanakhala kt akunena ndi atumbuka fine and gud,koma alomwenso adamva momwemo kt mumkat zitete.

 62. Ma pressident a2 ndiamenewa akt tixidya xitete nd mbewa ngat iyeyo angamadye xmenexo xopusa ngat amasowa xoyankhula osamangokhala bwanj!!! xausilu, xakachaso, xopusa, xamasile bas prexdent wanzelu aka liuxe xiko kt lidya xtete?? xausilu bas !!!!!!!!

 63. Vuto lathu a malawi ndi lakut sitimudziwa president wathu the he speaks zot samatha kulankhula chihewa zimaoneka ngati sitidziwa mwina timpezere interprater mwina zizaenda apo biiii mmmmm we wil stil have problemz wth him up to 2020

 64. zicheche ndiye chani asanamepo apa kumangot ophuzira kut apatu zamkhotha nkhuyu amalawife ubulutu opanda kuthirana kankhondo abale apeyaniya anafa onse kumangot la ntendere dzikoli zinthu zikupita

 65. Kutanthauza Kuti Amalawi`fe Sitivetsetsa Bwanji Osapepesa Anthu Munawasololera Misonkho Yathu Munaba Pano Mukukamba Motumbwa Bwanjinso? Mavutowa Akukula Chifukwa Cha Anthu Adyela Ngati Inu Ena Mwawelenga Mumuze Kuti Zinthu Zafika Chonchi Chifukwa Chakuba Kwawo.

 66. Amalawi penapake tzikhara ndiumunthu ngat anthu oops Mulungu,kodi makolo any kapena inuyo simudarakwitsepo,munthu ukat ulibe tchimo ndekut ukunama komanso ukungodzinyenga chabe,enanu ngat mumanyoza makolo any kuli bwanji President mungamupatse ulemu zosatheka,tphunzire kuremekeza atsogoleri athu posatengera chidani chosiyana zipani ayi,kumalawi mtsogoleri wadziko ndimodzi,sizidzatheka kukhara Ku atsogoleri angapo panthawi imodzi,ngat muli omvetsetsa musinthe,chifukwa mapeto akebe muyang’ana kwa iye ngat tata wafuko,ndale sitidya tpange zot titukure Malawi basi tonse ngat ana afuko limodzi,dziwani kut amene mutha kumufuna lero pamawa adzakharanso m’dani wanu akadzalowa m’boma,tmusiye Muntharika alamulire nthawi take,pamene zarakwika kungomukonza osat kumunyonza kapena kutukwana boma ayi,

  • ndipo amene akumunyozawo mtsogoleliwo machende awo @anthu basi kusiya kuthamangathamanga mmalawi muno basi kumakama za ziiiiiiiiikkkkkkkkkkkkkkkkkkk amalawi ambiri ndi makape kwambiri.pali munthu osalakwitsa speech polankhula ngati iye ndimulungu iyenso ndi munthu ndithu amavanso njala ngati inu.ok mwina magazi albino mukuwaphawo akupengesani misala eti? Guys pali nkhani zoti titha kumacheza koma sizonyoza mtsogoleli

 67. A malawi omwe muli kumuziko limbikirani kudya mbewazo ndi zitete poti walamura president wanuyo mwina ndikudzimaliza coz zimaboola ma plastic anyumba zathu maka ife timagoma manyumba amauzufe

 68. U better stop joke on serious things people there in pain…..shortage of food no enough electricity no medication…I steed of giving them hope then you coming with useless speechless…am always…feel shame on my country zikanakha zotheka kut president amabweleka tikanapepha azathu aku Tanzania kuti atibweleke MAGAFULI mwina Malawi akanasitha cz this 2 much

 69. Akunama ameneyu coz waona kut analakwitsa komanso anthu zikuwabhowa heavy chimodzmodz Bakili atanamiza anthu kut awagulira nsapato anakananso,kodi mwatitola eti?????

 70. ok ndamvetsa kuti anthu tinamva molakwikwa. according to his speech. zicheche tinamva ngati zitete. mbatata tinamva ngati mbewa. misquote tikumva ngati mosquito. nde Amalawi tizimuvetsa munthu wamkulu chonde please. what is required the President should have sn interpreter so that we should be getting him right.All in all there is hunger in malawi that’s why the President wanted to mean that we should have variety of food items.

 71. Dear Madam Calister,
  You know our problems in this country so we need your help please.You married to Mr Chimombo he passed away then you married to Bingu he passed away as well.So help us with this dude Peter,u gonna make plan poti mukuziwa kale mochitila mwake.

 72. Kodi ndi Mr jokes kapena kapena copyright ya kuchitekete kkkkkkkkkkkk wachedwa nazotu thabwala zakozo pano fans yatopa ndi ululu wamaluzi,njala,kuphedwa kwa Albino,kukwela kwazithu iwe ndiye uziselewulanso kkkkkkkkk ukunama hvy

 73. Amalawi penapake tatiyeni tizivomeleza,tikinziwa kuti munthu opanda mano kuti atchule liwu penapake amavutika.Ndidamva adati ZITETE koma mwinadi amati ZITCHECHE.Langizo kwa Mr president he must learn how to pronounce words properly kuchitila kuti angazatukwane pali chikhwimbi cha anthu.

 74. Malawians chimene amaona always ndi zofooka za president, bwanji timalephera kumayamikirako atsogoleri athu? Kamuzu takhala tikumunyoza; Bakili chimodzimoziso, Bingu tamutukwanso, Joyce chimozimoziso pano ndife tikumutukwanaso Peter. Kodi amalawi tizayamba liti kumayamikirako atsogoreri athu most of de time? Thus why dziko lathu silingatukuke coz eni akefe sitiziwa kumayamikira atsogoreri athu. Tizitha kumawamvesesa kuti nawoso amakhala ndizofoka zawo. Choncho tiyeni tiyambe kumanenako zabwino za atsogoleri athu omwe akutilamulira. Ngati m’banja pena zinthu zimatha kuvuta pena kuyenda; what about nation like Malawi?

 75. Malawians chimene amaona always ndi zofooka za president, bwanji timalephera kumayamikirako atsogoleri athu? Kamuzu takhala tikumunyoza; Bakili chimodzimoziso, Bingu tamutukwanso, Joyce chimozimoziso pano ndife tikumutukwanaso Peter. Kodi amalawi tizayamba liti kumayamikirako atsogoreri athu most of de time? Thus why dziko lathu silingatukuke coz eni akefe sitiziwa kumayamikira atsogoreri athu. Tizitha kumawamvesesa kuti nawoso amakhala ndizofoka zawo. Choncho tiyeni tiyambe kumanenako zabwino za atsogoleri athu omwe akutilamulira. Ngati m’banja pena zinthu zimatha kuvuta pena kuyenda; what about nation like Malawi?

  • Iwe Usandikwiyitse Zabwino Akachita Sukumva Kuyamika Ok Ndiyamikire Tikuthokoza Fuel Aliponse Ponse Koma Zomatokota Mofoyira Zatibowa Heavy Ngati Ndiwe Khadeti Umuwuze Amve Basi Kholo Lopanda Nzeru Ma Advisor Akenso Mbuzi

  • Kodi akutuma pitala muthalika eti? ? Iweyo ndithu mavuto ose ali dziko muno ungamati timuyamikile president? ?? Ulibe mzimu ase ngati president wakoyo wava.

  • Anthu ena ndinu opusa kwambiri, munthu ungayamike chiyani apapa. Mkulu wake adali bwino kwambiri 4 only first term. Koma term yomaliza adaononga zinthu kwambiri. Nde Chitsiru ichi changoyamba ndikuononga kokhakokha munthu ungayamikenji???

  • Kodi mesa amati voterani chimanga.Nanga izizoti indyani yamu ndi makoswe,ine ndidye zotisindinadyepo kamba ka khumba imeneyi?pa amake ndithu konse komwe aliko.

  • choyamba munthu wakoyo ana nena kuti zitete ndipo kaliyati anati ama joker lelo akuti ndimati yarm kenako zoyamika palibe mwava a mathewe chimene akupanga ndi kulemba mbava kupolice kukubweraku tidzakhala ndi mbava zambili police yose kuphatikizapo iweyo akungokoza kumwera uwone mene ililimisewu ku bts nd zomba ndiye ufanizile kumpoto mzuzu ndi lilongwe panopa ati akoza stadium pa zomba koma ndalama amadula tose uwerenge nyasa times umva chaponda mussa cashgate 577 bilioni kuphatikizapo munthu wakoyo

  • choyamba munthu wakoyo ana nena kuti zitete ndipo kaliyati anati ama joker lelo akuti ndimati yarm kenako zoyamika palibe mwava a mathewe chimene akupanga ndi kulemba mbava kupolice kukubweraku tidzakhala ndi mbava zambili police yose kuphatikizapo iweyo akungokoza kumwera uwone mene ililimisewu ku bts nd zomba ndiye ufanizile kumpoto mzuzu ndi lilongwe panopa ati akoza stadium pa zomba koma ndalama amadula tose uwerenge nyasa times umva chaponda mussa cashgate 577 bilioni kuphatikizapo munthu wakoyo

  • Samuel i think iweyo sunapite ku xool thus yyy sukudandaula za university fee think about our children mudzakwanitsa bwanji ngat panopa yafika pomwe ilipa?

  • mbuzi inu ngati uĺi ulesi izo nzanu mumati azikubweretserani chakudya patebulo kapeña kukulipiliràni fees kuzolowera zolandira eti?ma ARV mukulandira aulere fees ñso ikhale ya ulère uĺesi basi

  • zisiyeni awa ndi ma cadet. akanya mwano zimakhala kut zalowa, amabwera ngat njuchi. akugwilitsiidwa ntchito ndipo ambiri mwa iwo amakhala mbuli

  • iwe ndi galu eti? Anthu angajombe kuntchito kupita kokavota mcholinga choti ovoteledwayo azikhala ndi zoofoka??kodi mesa momwe timkadandaula kuti kuli njala iyeyo amkakana?? tamuuza kuti ife timadya makoswe akewo?? Nonse mbuzi

  • For a man of his status and calibre, use of sense of judgement and law of timing should be the order of the day. He should avoid making petty mistakes because he is more than just a public figure. Kuyamikirako ndiye tiyamikire zitizo? Vuto ndi loti everything is getting off hand including our worst enemy, corruption. The most unfortunate thing is, those within his inner circle are haunted with cashgate and will make sure that ACB does not prosecute…Tisoweranji umboni wina.

  • Vuto ndiloti wina akapanga develop challenge m’boma lero,people won’t face that challenge today but akazalowa wina nde amene amakumana ndi chivuto chija, Malawi sidzatheka mpaka kale even kutabwela president wachizungu,kaya wamtundu wanji, koma malawi will remains the good example of poorest country around the world

  • And I quote David Tramp, American presidential candidate: ……and there is a certain president in Africa who claims to be a professor who attained his studies in America but he is failing to maintain the economy of a small nation. You think high education is anything to do with good leadership??????

  • Kkkkkkkkkkkkk no , big NO. Can a professor leader leave the state house and tour an 800 m long of unfinished tarmarc road? Kkkkkkkkkkkkk

  • I can’t say ndiofooka so fast kapena kuti ndiwabwino, big No because our current kwacha was better that this what you call Rand,but today our kwacha is like a tissue,it’s not Peter, but we drugged down our own country, ourselves. Because of corruption,too many greedy leaders😀,lucky of patriotic😜,malawi sidzatheka ndithu, take a look at zambian kwacha today 😄😄😄

  • iwe Charles kulimbikila kumasamgalasa ulakhala ndi chiyembekezo.nanga munthu kubzala mbewu pa mwala nkumati ndikolola.

  • Point out just one gud thing that he is doing!!! Anthu are u blind? When u want to be a president be ready kuti uzanenedwa. U president is not for simple hearted aaaah!

 76. I voted for better living and now the same vote tells me to eat rats for better living what coincidence.
  I will start where my brother stopped. No strange.

 77. A Malawi enafe basi ndife okanika. Ntchito kulimbana ndi ma quote a President. You mean president it’s not a human to make a joke ? Some of us will die like that with full of enmity inside us. I am sorry for Malawi. Grown up people always ways depending on one man by the name of President. Do you think one man can change development of the country, eradicate hunger and end crime? Stop being king fools Malawians. Open up and start looking for a means of helping our country Malawi rather than quoting what president said.

 78. a peter zopusa ife ayi,ndifenso anthu oti timaganiza mwamva? muona ngati kukuvoterani kuja wamzeru ndiwe wekha? ife timakumvanitu mukamabwebweta pawailesi paja zopanda mutuzo ,ndiye osamanama

 79. If Ku mulanje tinakuumvani bwinobwiono bwana koma vuto atola nkhani ndi a opposition kujijirika kupisilira za eni kkkkkkkkkkkkkkkest

 80. Ur not fit for jokes & not fit to be a president even not fit to adress the public think wisely. Zomba central MP said dpp women danced for you empty stomach did u hear that, whats ur comment on that& YUNUS MUSSA MP for 2019 this is what u said with ur big mouth have you already casted ur vote for 2019? this is where ur stupidity is think before u speak OR choose AARON to speak for U.

 81. Kodi mbewa ndi zitete tiyamba kudwa pano? Ndani sakuziwa kuti wanthu ena amadwa mbewa ku mlw? Nothing to tok of zitete coz ambiri amadwa, what iknow is dat kholo likazingwa pakhomo limayesesa kuti mwana adwe basi nomata what kind of food simply tosave our lives. Taona ma shehk akudwa nkhumba mzimbabwemu akuti kukankha galas pa ngozi so what more mbewa and zitete?

  • Funso ndilakuti munayamba mwadyapo zitete pazokha nkukhuta? Kapena kuthetsa njala? Zikavuta mnyumba kholo lanzelu limafotokozela ana ake mowalimbitsa ntima osati mwachipongwe kapena ma jokes. Siriasly its nt fair kwa munthu amene anadya dzana mpaka lero angomwa madzi

  • bakili was only man oziwa kuti batiza nalo boza potembenuza mau ok. bt 4 u mr peter amalaw asukusula simungati thimbise nawo boza ok mwanama mr APM. kod mnyumba mukakhala njala kholo limatani?? kodi silimalimbikisa ana ake kuti pano zandivuta koma tiyen tipemphere mulungu sataya wake atithandiza!!!! lero mnyumba muli njala kholo mkumauza ana ati pitani kuthengo mukaphe zitete and mbewa!! wht typ of kholo is that??? tell me!!

 82. nde tilibe makutu kut sitidave haha wailephera ase ndi former President ekha amene amatinamiza and now tili ndi experience munthu sangatidoje wagwa nayo try again later

 83. Bola kukanakhala kuti ndi manyuzi pepala akumalawi okha amene alemba zimenezi but nkhani yoti amalawi azidya zitete ndi mbewa ili everywhere padziko lapansi. Zachisoni

  • Zoonadi aunt, inenso ndili kuno ku Tz ndaona mmanyuzi even mma social media osiyasiyana even beyond CCTV, NNV, Voice of Africa, African News ndi ena. Ndamva chisoni ndi manyazi mmene anthu akuno akulembera macomment awo.

  • Ndamalawi tikudziwa kuti ndamene analengeza that’s why tamvera chisoni dziko lathu coz nkhaniyi its everywhere and Poona aliyense akuyankha malingana ndi maganizo ake, ena akutukwana president wathu ena akunyoza mtundu wa amalawi, ena akuti mvera chisoni nde ndi nkhani yosakhala bwino ndinso yamanyazi kwa ife amalawi.

  • I’m in Nigeria n dis story is everywhere here its disgusting.Mr President must learn how to pronounce words properly other wise he will mention privates parts one day

  • # Joshua Ganizani Mukutantha Uza Kuti Alendo Ali Kumalawiko Sakumva Chichewa Bwanji Iwe Ukuyika Kumbuyo Chindele Ndi Ofoyira Adao Anaba Ndalama Zambiri Zamisonkho Pano Azitokota Mopusa Ndi Kape Ameneyo Wasowa Mfundo Nkhaniyi Yafika Ku India Komanso Uk.

  • Kodi iwowo poyankhula zimenezo mchilomwe, amalekelanji ku translate patsikulo? Ndangati anthu amatha chilomwe ku Malawi even anthu aku mulanje, phalombe even thyolo ambiri samachidziwa. Pano nde akuti amathanthauza yams , ndi bodza. Tayaluka basi amalawi ndi mau ochokera mkamwa mwa president wathu.

  • Ine ndili ku Brazil nkhaniyi kulibe moti ineyo ndaiyimvela pa fb pomwepa. Koma vuto timakhala anthufe timakokomeza nkhani kwambiri nkuona timapha anthu amoyo nkumati amwalila pomwe lili boza, kodi ndi president uti sananenepo zolakwika ku ntundu wa a Malawi??????????????

  • Ine ndili ku Brazil nkhaniyi kulibe moti ineyo ndaiyimvela pa fb pomwepa. Koma vuto timakhala anthufe timakokomeza nkhani kwambiri nkuona timapha anthu amoyo nkumati amwalila pomwe lili boza, kodi ndi president uti sananenepo zolakwika ku ntundu wa a Malawi??????????????

  • Iwe Mike Mvula kodi ku fb unangokhalapo ndi cholinga choti uzingokomenta pic za anthu or bwanji? Ngati umatero ukutsalira kwabasi popeza anzako tinàlowa fb kuti tidzidziwa zochitika zammaiko osiyana siyana. Like manyuzi, TV even magulu osiyanasiyana uzionere wekha usangoyankhula. The news is everywhere.

  • Ellace Chirwa pali ma pages ena pa fb athu ena samawawona,, nditakufusa fuso limodzi dzoti nduna ya za chuma kuno ku Brazil yakana kepereka ndondomeko yazachuma munyumba ya malamulo chifukwa choti wayambana ndi nkazi wake nkhani imemeyo pa fb wayiwonapo????

  • Iwe mike mvula kodi BBC, News of Africa or How Africa. Com, CCTV, Voice of Africa, BBC Africa, Aljazeera zili mdziko limodzi? Kodi uli world it iweyo ya technology or yakale? Ndakudabwa kwabasi. Ine ndikukuuzane ndili kuno ku Dar es salaam and nkhani zimenezi ndazionera mma news nde iwe uziti uli ku Brazil, Brazil wake uti opanda zimenezi. Tseguka mmaso and udziwe kuti Malawi wayaluka from now ndi kunyozedwa komwe makamaka president wathu ndi macomment aanthu. Ngati sudziwa mmene tingamajoinile pa zinthu ndatchulazi ndi bwino ufunse anthu ozindikira akuuze mmene timachitira kuti uziona zambiri. Open your eyes Mike!!!!

 84. Nkhawa Free Bwana Presient Akusowa Chokamba Anthu Olephela Yawo Ndi Nsanje. Ine Ndinakumvesesani, Mulungu Akudaliseni Pamene Mukuyendesa Stima (Malawi) Ikakhala Nkhani Ya Zatchuma Mako Ambiri Akuvutika Amene Akulamulila Kumeneko Sindinu Bwana,

 85. Thanks Professor for the clarification. I hope, at your pleasure, you shall also clarify on ” mbewa.” Am sure you also meant something else on this word. Am sure you did not mean MICE. Kaliati clarified that you used the words but you didn’t mean it, YOU were just cracking a JOKE. I think you may wish to clarify this to her during a cabinet meeting. This problem of misquoting the President, the most learned professor, the most ELOQUENT SPEAKER, THE GREATEST ORATOR must indeed stop. My suggestion is that DOCTORS should PROVIDE EAR TREATMENT/CHECK UP to all citizen, starting with journalists.

 86. ALL US TIZASOVA TIKAZAGWA NDI NJALA IN RSA ANASOVA KALE MOKOPU KUPANGA NDIWO (maungu,mphonda,mango osinjansinja alongside mapeyala)INE NDADYERAPO NSIMA LIFE KUMAYENDA PA JOZI

 87. mukutionjeza Mr Peter kodi munayakhula chiyakhulo chanji???? mpaka anthu osakumva koma ndi mzika yeni yeni m’malawi muno.

 88. Nditsatse nawo malonda pano. Ndili ndi mankhwala oonjezera mphavu za abambo kubedi, kukuza chida cha abambo, kukuza/kupepetsa mabere, m’bweza nyini, hip booster nnzina zambiri

  • akongofanana ndi mugabe koma nde mubwiladi zitete bas coz mugabe xizinthu angodikilila kuzima basi kuthawa milandu

 89. Malawians We Have To Learn Respect To Our President,kodi Ngati Tokhatokha Tikumunyoza Mtsogoleri Nanga Anthu Amaiko Ena Amulemekeza Bwanji? Kodi Nthawi Ya “Kamuzu”zimenezi Zinaliko?

 90. Don’t think you are talking to your children,you are full of stupidity,galu,nkhumba this is not time for jokes . People are seriously looking for your help(mainly hunger crisis)and you are talking rubbish.If you want jokes do with your step sons and daughters in your house……..i hate you.

 91. …and he didn’t say mice but rather minced meat. This reminds me of Bakili Muluzu who refuted the claim that anati azapereka fetereza waulele ndikunena kuti anati fetereza wa urea.

%d bloggers like this: