
Tough times are upon Malawians following the announcement by the Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) of a hike in fuel prices effective midnight, 10 June 2016.
Mera has announced that Petrol will sell at K788.30 per litre from K743.30 representing 6.05 percent increase.
Diesel will be selling at K766.90/litre from K 722.80 representing a 6.10 percent increase.
Paraffin will be selling at K609.80 a litre from K580 representing a 5.07 increase.
187 thoughts on “Fuel prices up”
Comments are closed.

Hlw amalawi
Zawonjeza Malawi mavuto osatha kalanga ine ndithawira kuti azanga
Palibe vuto ngati kuno Ku South Africa fuel wakwera katatu mondondozana pa mwezi iwiri yokha ndiye akanene kwathuko ku Malawi
Time for the Light is coming!!!!When there shall be no any sorrow.The whole world under one government!!!United world.Under one King(The Light)!!!.No poverty!!Cnt wait to see it coming.
u will never see that dark one world gorv. in ur life time
Its all over de world guys
Zachita kukwela nkoko kowengako,, muzizisata kaye osamakobwetuka apa,,,
Even here in RSA wakweranso palibe chodabwitsa apa
No where to go and no-one to blaim lets kp 4ward gentlemen, hopefully God ‘ll fight for us.
WINA DZIKO LIMUKANIKA KAYA. RUNNING A GOVT IS INDEED SERIOUS BUSINESS.
kulikonse Mafuta akwela inu koma umbuli onyoza boma udzatha ena mpaka maphuzo ndithu chonsecho olo galimoto alibe mkomwe u savage basi
By the end of apm term we shl buy pt at 2000,dz at 1700,pr at 1500,or more bliv it or not
nde nafe tikwezeso ama minbus
Ku RSA anakweza last week ndi 70cents /ltr nde tisamude wina kulikonse akwexa basi
Malawi suzgo pa suzgo.
Malawi suzgo pa suzgo.
Kukwera kwa FUEL sikuMalawi kokha nde sivuto lamunthu
Boma iloooooo !
ndiye a Kabanzanso tikweza ndi 50%
nanga dizilo
Zili bwino mafutawo samapangidwa mdziko lathu ndiye tikufuna profit yoti tikaodelenso