Micium Mhone chased in Flames camp

178

Flames and Jomo Cosmos winger Micium Mhone has been sent home by Coach Enerst Mtawali due to indiscipline and has since been replaced by Mighty Wanderers winger Isaac Kaliyati,Malawi24 can confirm.

Mhone refused a handshake with Muhamad Sulumba when he was substituted by his coach during Malawi’s 3-nil defeat to Zimbabwe in the Group L 2017 African Cup of Nations qualifier on Sunday afternoon.

Micium-Mhone

Micium-Mhone sent packing.

Soon after the game, Mhone wasted no time by taking to his Facebook wall where he vented his anger on Mtawali’s led Technical Panel.

This did not go well with Mtawali who immediately dropped the former Blue Eagles winger in his squad for the Cosafa tourney slated for this weekend.

Mhone jetted into the country from Harare some few hours ago via Chileka International Airport.

Meanwhile, Kaliyati is expected to join his team-mates in South Africa before enrooting to Windhoek where they will play Angola in the competition’s opener on Saturday.

After the game, Mtawali made a public apology to Malawians for the defeat saying he will now target the Cosafa Castle Senior Challenge Cup to console the nation.

Share.

178 Comments

 1. uwu simpira koma mwayi wa ntchito tazingo yenderani mayikowo bola mukulandira on time ifenso kuno tikupanga zathu mungangotichedwetsapo apa

 2. Iwe Enerst Mtawali, ife kuno tili ndi mkwiyo kwambiri kuposela mkwiyo umene iweyo uli nawowo, ndiye linda mazi aduse kuti uziti ndiwedi coach wa Malawi national team. Utipeza ukamachoka ku Namibia kwakoko ndi team yako ya Bullets watengayo.

 3. mukungonamizana apa flamz yacntha kangat macoach,,? ndie cidacnthak ndician,? cot muziwe kukhal mmalawi ndikulimba mtim olo zitavuta buanj flemz czathek that y ineo ndidaitaya palipose mot iney flemz ikaluza ndimasangalala sikufuna kom kut flemz imaonjez

 4. Tingomukhululukira mtawali nthawi ya unyamata wake anadya chamba kwambiri nde pano decision imamuvuta kanundu uja ndi waukali

 5. Micium ndiosalakwa vuto anatopa kumamenya mpira ndima coach osathandizawo mutawali amakanika Ali player ndiye panopa azitumbwa nyani wachabechabe timangooneka ophweka ikani ma coach ake timangosankha mbewa

 6. This ernest mtawali is very clueless when it comes to management you mean to tell me kaliati is better than mhone???is namwera better than ng’ambi??hes treatment of the senior players is uncalled for and if this is going to continue he is asking for trouble

 7. Ndekutiso mu ground mukumafunamoso displine nchifukwa chake mukuluza. Tadzingoluzani bola mukudya ndalama zosapindula nazo

 8. What did you expect from a boy playing in a relegated Jomo Cosmos, thats why some of our players amalephera kupita patsogolo, khalidwe nchuma n mpira ndi masewero Mhone n Kinna once said’their is no permanent position/place for someone in the field of play/ground.

 9. Why uddnt chased out all and gave zim free poits than to play nyasi ngati zimenezo? Who gave u coach ? Pack& go timaluza inde koma iweso wanyanya kubalalisa team

 10. Mtamali ndi opoira mwana uja atalowa sanayenera kumutulutsa . Mkona zinamunyasa , game imeneija anayenera kututsa Chiukepo sanali bho . Micium tamulandira . Mtawali ndi team yako musabwerenso kuMalawi .

 11. Rex Amon umbuli osamaubweletsa APA. Let’s talks about football and don’t insulting other tribes. If your head is empty just keep quite. Munthu wanzelu salankhula ngati alibe cholankhula.

 12. Ngat coch waona kut iyeyo sakusewera bwino amafuna azingomuyang’ana? Indicipline imapangitsaso kut framez iziruza akuziva chani Micium yo mu2 wot bench ndibwez lake bwanji sakwiya osangothokoza kut anamenyako 15min pa Malawi pano saliposo yekha player ndipo asazaitanidweso ndiopanda khalidwe chifukwa chot mwayamba kumenya kuja mukufuna muziziva? Zopusa bas mxiiiiiiiii

 13. For the Love of the Flames Often I feel the need to comment on the National Football team’s misfortunes but seldom do I have the energy to begin to write. Where do we start? Are the Flames indeed a “Load of Rubbish” as one Anonymous Times Reporter puts it? Is the problem with the National Team the National Team? Are our expectations of the Flames realistic? Often these questions are left divided in opinion. I do not think calling the National Team a “Load of Rubbish” is a sensible or fair argument. We supporters call for change every time the team performs badly. We call for management change then squad change then government reform all in the name of hoping the team plays better. We want success instantly. We want to see a group of old tired souls gallivant the field in one last hurrah, defying age, time and most importantly statistics. To conquer the the continent against all odds and bring pride to a national that would careless about their success. My opinion, Malawi has potential. Choose whatever football model to learn from, Spain, Ivory Coast, Leicester or maybe even Brazil. The fact remains, Attitude, Discipline, Continuity and Belief wins titles in the long run. Give the team time not pressure. After all we won’t be able to pay for the teams travel expenditures. # justsaying All for the love of the Flames, or whatever is left of them. “Believe in your potential even if you haven’t seen the results”

 14. Discipline…..??? Kupha team kumeneko…..coach ozitsata amangotsanzika basi…. Mtawali asaone ngati vuto sitikulidziwa….Mtawali must go!

 15. Micium mhone is one of the most disciplined member in the team and it was an insult just to play him 15 mins from the bench and sub him off.Ernest Mtawali is a clueless coach and he must sacked soon after the cosafa

 16. Discipline imakhalapo mukamachita bwino koma ngat tikumangoluza luza pakhala bwanji discipline? Nw wathamangitsa player wabwinotu apa ife sitikusewelera discipline mpira ayi bola kuwina magames basi taziyesesanikoni nthawi zina

 17. nkhani za mpira ndithu ungadwalenaz…. coz coach safuna kt azuzulidwe?? safuna kva malangiz a athu?? tikadali kuluza mpaka kmwe ku cosafa??

 18. Micium Mhone sanalakwise Enest Mtawali sakuziwa ntchito yake azingomwa kachaso bac asatiyalutsile team inde Flames imaluza koma simbuzi akupangawu

 19. Chofunika ndikuthamangitsa mtawali asiye zampira komanso achoke mmalawi komanso passport ya chimalawi amulande kuwonjedzera apo katundu wake. Ndi nyumba zigulitsidwe ndalama akawo ede anthu odwala Ku chipatala

 20. Mhone mukuzipopa chani siinu nomwe mwabwelera ku FND Ndiye dziko likawine coach mutu wakenso sukugwila kusiya achina Ng’ambi akumenya every week.

 21. Mtawali akutengera maina zoona.Wadabwa he is not a nation team material.Silver inamutaya ku johns anamutaya pano mukuti ndi sticker wa nation team,very strange.

 22. Vuto la malawi national team c mtawali ai ai ai. Ndakana kod vuto loluza layamba nd mtawali? Kwa choka ma couch angat?
  Khani nd preparation yanthu imakha yodulira, komaso bwezi titayambila patali under 20 , 23 komaso waste department kwambili nd fam kholo la mpila palibe chomwe akupanga atule pansi maudindo aka matula mtawali iwonso asadzike

 23. mpira ndiosiyilana palibe cholakwika ap. mtawali wachita bwino for send him home. Alibe khalidwe player ameneyo

 24. Better being chased than being called in this so called failure camp,,,,better be associated with indispline than shaming urself in the name of flames squad,,,,,,chase them all for indispline and see urself holy in puting insults to our beutiful nation,,,signs of kulephera umapezera zifukwa ena,,,,waiting to eat money again??we will still poorly contribute for ur survival though with tears.

 25. MECIOUM IS NT THE PROBLE BT THE COACH HIMSELF…..HE IS FOND OF FRUSTRATING UP COMING PLAYERS AND NOW WANTS MECIUM TO BE ONE OF THE FRUSTRATED ONE…..BT HE MUST REMEMBER A PLAYER REMAINS A PLAYER UNTIL HE IS OLD ENOUGH TO RETIRE WHILE A COACH CAN BE CHASED OUT THOU HAVING A CONTRACT……NTAWALI NOW WANTS PEOPLE TO TALK MORE OF HIM…….

 26. Mpira umenewu utionesa zinthu Komanso uwusa mapiri pa chigwa. Kenako tidanapo .mwachitsanzo , taluza chifukwa choti munadzadza atumbukawo akukonderana polowetsana ku National team. Pepani ndangodutsamo mzocheza izi .

 27. Nothing Can Change Even Titabwerekera Achina Wenger, Morinho Flames Siidzatheka Basi I Dont Want To Hear The Flames News Again Zikutipweteketsa Mutu

 28. I don’t have problems with Mtawali’s decision. Mecium’s conduct following his substitution was regrettable. However, this should not be infinite.

 29. Mtawali shame on you, laugh at him ha!! ha !!ha !!ha !!The only result that Mtawali has produced is descipline. Whats the point of having a team full of desciplined players but which doesnt produce any result. Mtawali how are u going to descipline players wen u are not desciplined yourself?

 30. Mtawali shame on you, laugh at him ha!! ha !!ha !!ha !!The only result that Mtawali has produced is descipline. Whats the point of having a team full of desciplined players but which doesnt produce any result. Mtawali how are u going to descipline players wen u are not desciplined yourself?

 31. Mtawali shame on you, laugh at him ha!! ha !!ha !!ha !!The only result that Mtawali has produced is descipline. Whats the point of having a team full of desciplined players but which doesnt produce any result. Mtawali how are u going to descipline players wen u are not desciplined yourself?

 32. In as far as discipline is concerned he deserves it! Mecium should know that talent & discipline make greatest sportsmen!

 33. Panel yathu si ili bwino, Mucia Mhone sanalakwe wachita bho wauza wise substution samatha coachyu kuma2lutsa ma midfielders nd kulowetsa ma striker mulu mground zomwe zinali zopanda nzeru. Coach mbola uyu….

 34. frankly speaking antawali mmaendela maina osatibamene angathandidze dziko,mmene ma player amaphonyela muja ana wadabwa osawatulutsa koma kulowetsa wina pompo kuntulutsa? zamanyazi mmene amasewelela mpila ngati aku ndi ana? ndazimvela chitsoni kukhala mmalawa nkofunika kupilila osati masewela, azitsogoreli anthu ngolephela kuchokela ku ndale mpaka mpila….dont stop me kulilaku….

 35. Ine za flames n’dachosa dala pano napanga ubale nimasendesende basi chifukwa ninaiona flames simanifunira zabwino izanipha ndi Bp imene ija ikagwere

 36. Now chase Mtawali too…he has been indiscipline since he started…loosing has been his new carrier, that’s being indiscipline too

 37. Palibe chimene walakwitsa.coach odana ndi maplayer a bwino choncho Malawi inga wine.kodi simuchita manyazi akakuchinyani? ntchito basi kumadyela ndalama maplayer kuti amenye game.coach ochititsa manyazi dziko coach wanji osakochako club kungofiki national team.ndankhumudwa nawe MTAWALI.

 38. Mtawali ingoyambitsa fellowship basi flames uthese ukutidwalitsa nazo mutu. Nanu ma players mukumangobonga game yomenya ndi amuna anzanu kaya mwatani. Kulemedwa

 39. its apity that we Malawians stll trust the same adminstrators that r destroyin our football…..the affliates that voted for Myamilandu again rily killed us…..see now we r regreating. five years tym from now flames will b totally quenched to nothing

 40. Coach waukape, mbanje inampweteka, satithandizanso, bwerako Micium , musiyile mbola zakezo, koma choti adziwe pobwela yathapo,apakile!!!!

 41. Zausilu bax #indiscipline_indicipline_chan???? Celebrety amakhala wamwano kumene …atengeni amakhalidwe abwinowo akapita kunja m’ground azingoyang’ana mages….kkkkkk IWE MTAWALI WABALALIKA IWE….FORMER PLAYER TO COACH……KKKK MALAWI

  • iwe sunaonele mpila ukanadzimvela chisoni kuona mmene anthu amaphonyela ndati axhita kuwatola panjila osati ngati ma player ampila.

 42. micium mhone is better than kaliati..discipline does not play football.zomwe anapanga mtawali palibe player amene angasangalare nazo,mhone sanalakwe.i enjoyed the game though.pitiliza kuluza mtawali coz ukatelo enafe timakondwa

  • Amwene Ngati Mumadana Ndi Kaliat Amenewo Mavuto Anu Chot Muziwe Nchot Athuwa Amasewela Malo Osiyana Ndipo Simungawafananize Ngati Ntawali Analakwisa Si Bvuto Lakaliat Umbuliwu Pemenapake Tiziubisa

  • what u said is total nonsense prince..micium mhone is a right winger/kaliati is a right winger.ask everyone else,mhone is better than kaliati& its uncalled for coach kumutaya kutenga kaliati.nkhani ya discipline osamayitengera pamgong’o.what mtawali did was stupid.the last time i saw that sort of thing happening in the english premier league was way,way back like 5 yrs ago.player kumulowetsa& kumutulutsaso within 15 minutes.ma player amakhalaso ndi ulemu wawo sitingamuyikile kumbuyo mtawali.sakho reacted furiously when he was substituted when liverpool was playing chelsea in the epl koma anali atavulara& anayamba game.imagine how mhone felt

  • discipline is important whether we lose or not i hope mukudziwa za benzema kuti sakumenya nawo euro ikuyambayi coz anamupeza ndi mulandu omwe iwowo ku france akuwutenga kuti zikhoza kuipitsa image yadziko mlandu omagawa pa porn video a player mzake

  • discipline is important whether we lose or not i hope mukudziwa za benzema kuti sakumenya nawo euro ikuyambayi coz anamupeza ndi mulandu omwe iwowo ku france akuwutenga kuti zikhoza kuipitsa image yadziko mlandu omagawa pa porn video a player mzake

  • &i guess u knw what the word discipline mean?nkhani ya litigation ndi discipline ndiyosiyana.am not saying discipline ndiyosafunika but dont over emphasise it

%d bloggers like this: