Man who married 14 year-old girl jailed for rape

184

The Ntchisi first grade magistrate court has sentenced an 18 year-old man to six years imprisonment with hard labour for raping a 14 year-old girl.

The court heard that the convict raped the 14 year-old girl at Mdzuche village T/A Chilooko in the district.

CourtAccording to police prosecutor Fred Luhanga, the convict, Willard Paul, went to the girl’s village and took her as his third wife without the consent of the girl’s parents.

But after two weeks  the community policing members  were informed about the issue and they took the girl back to her parent’s house.

In mitigation the convict told the court to exercise lenience when passing the sentence as he has a sick mother at home in need of his attention.

But first grade magistrate Dorothy Kalua said Paul deserved a custodial punishment to deter other would be offenders.

She sentenced the convict to six years imprisonment with hard labour for difilement, an offence contrary to section 138 of the penal code.

Paul hails from Dzutche village T/A Chilooko in Ntchisi district.

Share.

184 Comments

 1. Kodi mundende zanuzi muli ndichakudya chokwanila ett,mungomanga ndianthu osalakwa.M’malo mot muzilimbana ndianthu amene akupha ma alubino mukumat mukawagwila nkumawapatsa zaka 3,4 km awa size imodzi mukuphera tsogolo mnyamatayu,kugwililila mumakudziwa km??banja limenelo atati akalambilane angayambe kukalamba ndani?zaaaziiii….!

 2. Hahaha zikanakhala kuti mkaziyo wadzaka fotini atamukwatilayo ana mung’amba bola koma damage palibe aaaa!Ndiye mutikwizinga ambiri chifukwa nanenso ndi kufuna kuzula wa dzaka 13

 3. Stupid thats not fair 6 yearz okuba aja bwanji mpaka lero palibe chilichonse pankhani ya cashgate km kumangotipweteka pa tax mwezi uli onse kukweza thats bad.

 4. Sometimes when commenting, we need to have constructive arguments. Otherwise we might end up showing that we are not conversant with our own laws that govern our country. If you go to marriage act, you will find that a boy or a girl should reach 18yrs when s/he is capable of entering into marriage. Any age less than 18yrs is taken as not mature enough to make decision own his own.

 5. Sometimes when commenting, we need to have constructive arguments. Otherwise we might end up showing that we are not conversant with our own laws that govern our country. If you go to marriage act, you will find that a boy or a girl should reach 18yrs when s/he is capable of entering into marriage. Any age less than 18yrs is taken as not mature enough to make decision own his own.

 6. Eish am 18 yrs old nde ndinakwatila nkazi wa 16 gv yrs panopa ndikufuna nkamusiye asanandiyimbe mlandu wa rape sinanga sindingakwanitse kukhala naye 2wks osamugona

 7. Eish am 18 yrs old nde ndinakwatila nkazi wa 16 gv yrs panopa ndikufuna nkamusiye asanandiyimbe mlandu wa rape sinanga sindingakwanitse kukhala naye 2wks osamugona

 8. kufika poti akwatilane ndekuti zinayamba ndikale poti atsikana amasiku ano sakumachedwa kulowa banja akangowona kuti kumaliseche kwawo kwayamba kumela msipu akumati basi ndakwana nde mwati amumanga chabwino poti ndimalamulo komaso atsikana amatiyambila dala ine kanachita kubwela kokha kena panyumba moti katafika ndinakalowetsa munyumba kamanamizila kuti kakudzapempha mchele koma nditawona zomwe kamachita ndinazindikila kuti sikamafuna mchele weniweni koma uchi uchi ee ndinamwa madzi ka zokugwa zokha sitizileka nde pomanga kumawunikaso pena atsikana pano achita chiwewe

 9. Kmano penapake 18yrs 3 wifes masanje chiyani?kpna ngwandalama kwambiri,paja akazi mmangokopeka mzaziii zomwe,mwina ali mkaokala,ndiye amangonyengerera mtima sweet kkkkkkk

 10. Can some one tell me the difference between Rape and Marriage? Is he a man or a boy? I understand the guy is 18 years old and he has already 2 wives plus that girl being a third wife, does this make sense? How old was he the time he married first wife? . The Malawi I know someone marries under marriage age gets 6 years other stealing Millions of Kwachas or Dollars and those found with human parts or killing albino gets less than 5 years . Really what is going on in our country?

 11. Hahaha even if its protection of a girl child, 14 against 18, and 18 is a male, i see blurr in the jugdement your honour show some leiniency, or protect both

 12. What About The Parents Of The Girl They Should Also Be Charged Coz Its Their Responsibility To Look After Her And Again The Punishment Is Harsh To The Boy Coz He Did Not Force Her Into Marrying Him She Did That on Her Own Free Wil

 13. What About The Parents Of The Girl They Should Also Be Charged Coz Its Their Responsibility To Look After Her And Again The Punishment Is Harsh To The Boy Coz He Did Not Force Her Into Marrying Him She Did That on Her Own Free Wil

 14. Kkkk..this has nothing to do with rape “Mr judge” ndizawana izi..komatu Malawi police mukutionjeza mwanva!! Mpaka 6yrs imprisonment?? Koma akanakhala a cashgate ndi ma albino killers ikanakhala less than 3 yrs.. Eeesh!! Chilungamo chinatha basi..

 15. Kkkk..this has nothing to do with rape “Mr judge” ndizawana izi..komatu Malawi police mukutionjeza mwanva!! Mpaka 6yrs imprisonment?? Koma akanakhala a cashgate ndi ma albino killers ikanakhala less than 3 yrs.. Eeesh!! Chilungamo chinatha basi..

 16. Ngati ndikumanga muzimanga makolo Bz they have all responsibility to they children, and they are ones forcing their daughters to get marriage before their age

 17. Ngati ndikumanga muzimanga makolo Bz they have all responsibility to they children, and they are ones forcing their daughters to get marriage before their age

 18. poti walakwira lamulo alandile chilangocho koma fuso langa ndilot wina anaba ndalama za amphawi mamilion komwe ndikupha kale akupatsidwa zakka zisanu zokha .chilungamo palibe apa nzanga wosaiuka pewa zinazi ungazafere kundende.

 19. poti walakwira lamulo alandile chilangocho koma fuso langa ndilot wina anaba ndalama za amphawi mamilion komwe ndikupha kale akupatsidwa zakka zisanu zokha .chilungamo palibe apa nzanga wosaiuka pewa zinazi ungazafere kundende.

 20. uchisiru siuposa pamenepo, mmalo omwera mowamu tikumapeza ana a zaka 11 ndi 12 akunyekhulira azibambo azaka50 ndiye inu mukumanga uyu wa zaka 18 ?

 21. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkk mukumumanga munthu chifukwa choti wadya katundu wake? Aaaaaah tathanani ndiza albino kaye osati muzithatha ma chance zausilu eti” palibe chifukwa apa

 22. Palibe man apa ana wokhawokha awa mmalo moti tipexe njira yothana nd anthu amene akupha abale a ch albunowa tixichedwa ndkumangana ukwat wot makolo a anawa avomelexana its waste of time

 23. Palibe man apa ana wokhawokha awa mmalo moti tipexe njira yothana nd anthu amene akupha abale a ch albunowa tixichedwa ndkumangana ukwat wot makolo a anawa avomelexana its waste of time

 24. Nde mwati 6yrs in jail with hardlabour?? U mean that case is morethan cashgate?? M’mayi ujayu 5yrs only, pomwe mwanayu 6yrs??may God 4give u judges.

 25. Pali Zomangirana Apa Akati Banja N’chiyani Ngati Pali khani Ina Nzoveka Koma Ngati Ndimeneyiyi Mutulutseni Akapitirize Banja Mmagwiritsa Ntcito Malamulo Pa An2 Osauka Bwaj Amene Mukuwadziwa Aja Bwaj Adakwatira Mkazi Oti Size Kukana Katsekeleni Kaye Amene Aja Osat Zopusazo

 26. 18-14=2only!!mmmmmmmmm nde mukuti”nzibambo wazaka 18 wagwilira mwana wazaka14??” mmmm Sizimasowa dziko likakhala m’manja mwa ana alucifer.

 27. That’s why we ve a lot of broken marriages in our rulal areas coz kids are forced to marry ve kids then later realise thy r not ready for marriage n thy pack their belongings taking the kids with them to be raised in their parents homes n it’s normal for them n it’s going on n on.instead of allowing kids to grow up n be ready for marriage thy r encouraged it’s ok to get married at 14 yhooo wonders shall never end in Malawi as long as am alive no one wil Marry my Dota at 14.the parents are very much at fault in this coz if thy didn’t want the marriage or if thy knew it was wrong thy shud ve protected their Dota from the marriage n no one wud be in jail for rape now the parents who allowed it are comfortable at home while the young man who married the gal with the concernt of the parents wil languish in jail,in such cases even the parses shud b brought to book thy allowed it for their own gain.gals are being turned into taking over the parents responsibilities at a young age coz parents feel the son Inlaw wil provides one or two things for them it’s just pathetic

 28. Izi nde zopusa realise the man from prison did he pay lobala to the bride? If yes inu sindinu oganiza munamumanga munthu mtulutseni mamuna akapitirize banja lake eighteen,fourteen zaka four zokha anasiyana it’s good match u judge what u did it’s ridiculous tsk!

 29. Judge yemwe wapereka chigamulo chimenechi ndi wachamba . Wakuba k105 milliln za boma kupatsidwa 5yrs pamene wina wakwatira mkazi wake 6yrs chamba eto?

 30. Pa Zakazo Amafanana, Nanga Mmafuna A Kwatire Wa Zaka 20? Kumaona Kaye Zinazi, Akuluakulunu Mmakwatira Nkazi Wosiyana Naye Zaka 25, Ndiye Kuti Mmapanga Defilement, Simuwamanga Bwa?

 31. Onsewa ndikaonesetsa sakukwanila kulowa m’banja chifukwa zaka zawo sizikukwanila pa malamulo an2 ndye apa plibe chifukwa choti apolice munene kti nyamata wagwilila. Mubwerereso kumene kwachitika khaniyi mukafufuzeso kawili. Ine ndikuona kti pli kusavana pkati pa mabanja awiliwa. Ndye mnyamatayu asakhale m’mavuto khani yake imeneyi. Chonde apolice fufuzana bwino monga mwantchito yanu

 32. A police aku malawi ndizitsilu amumanga bwanji ndikumutchaja zaka zonsezo pomwe wina dzana lomweli wina anaba ndalama za boma zokwana K105 million kumutchaja 5 years osatiso hard labour km inu!!! Muzandilakwitsa

 33. Simesa onse ndi ana mamunayu anali asanakwane 21yrs winayu anali asanakwane 18yrs, ndiye pali man apa, osamanga makolo awo bwanji, kumalawi ufuluwu mwangowakhuthulira azimayiwa ife ndiye tilibe ufulu et?

 34. Simesa onse ndi ana mamunayu anali asanakwane 21yrs winayu anali asanakwane 18yrs, ndiye pali man apa, osamanga makolo awo bwanji, kumalawi ufuluwu mwangowakhuthulira azimayiwa ife ndiye tilibe ufulu et?