Tay Grin is not the best rapper in Malawi-Martse

Tay Grin-Chipapa
Tay Grin-Chipapa
Tay Grin not in Martse’s list at all.

The Mwano hit-maker has been rocked in another spark of controversy having recently crowned the duo of Gwamba and Krayzie G as best rappers in Malawi, against the collectively held belief that Tay Grin is the king of local hip hop.

Martse created a debate on social media yesterday having posted that the said rappers are above the rest in local hip hop.

Martse
Martse his list has earned him trouble.

While others supported his position, others labelled it ridiculous that only a drunkard like Martse can have such a lame opinion.

The debate seems to favour the opposers who have unanimously rained all sorts of sin language against the Natural Resources College student.

However Martse does not seem to be moved with what others think about what he thinks, after all Duncan Gwamba Gzambo, and Phineous Krayzie G Moyo are his good friends.

This comes amidst claims that local urban artists deliberately make controversial posts on social networks so as to attract media attention.

It is believed that most artists have the truth in mind but opt for the opposite on social media networks.

Advertisement

616 Comments

 1. Aftr de ril elements malawi’s hip hop international aftr them came nyau king,kod achina matse,gwamba,dictator,u name them amaaziwika abroad??…..can they stand de hit internationaly

 2. Guys Rapper amene amaziwika kwambiri ndi Tay grin ,enawo ndi ammakwalala ,mupite ku southafrica ,Zambia ,german ,Belgium,america ,amamudziwa .chifukwa chani akati oyimba oziwa amatchula Lucias Banda?answer chifukwa ndi Otchuka komanso ali ndi zochita ,amapeza ndalama .Inu makashuta ka music video kanu ndiye kuti ndi ka Five pin .Go to hell brother sunafike kikkkkkkkkkkkK

 3. A Malawi 24 akumazandinyasaso penapake!!!! We call something News if it has an element of unusual….nde zomati muzitidanitsa aMalawife sitikufuna……u are just a bunch of rubbish……

 4. Kumeneko nde kusonyeza2 umbuli wako onse gwamba,kraz g marapr uchitsiru eti ndan sakudziwa ntchto za 3rd eye D kalilan awa nde makina gwamba,krazy chbwana eti ana onyeranyer asazifanizle nd tay g

 5. Kumeneko nde kusonyeza2 umbuli wako onse gwamba,kraz g marapr uchitsiru eti ndan sakudziwa ntchto za 3rd eye D kalilan awa nde makina gwamba,krazy chbwana eti ana onyeranyer asazifanizle nd tay g

 6. Akape Amartse chifukwa chofananitsa nkhaka ndi kaimbi akumatha kuona ngati mzithu ziwiri zofanana,Tay Grin ndi rapper bst than kamwana koonda ndi mowako ka Crazy G ndi wamutu opanda longtudes Gwamba mumangoflowa zomva nokha basi bola mental yabo,mukaimba nchichewa sizimamvekanso tamvani aka Ha chipapapa papa zikuwawa coz zawo ndi national level komanso samagudwa makape ndayakha bif atleast,mxiew

 7. Grin amatha enanu yakula ndi nsanje basi, Ka martseso ndi kachiani? Tay grin wadutsana ndi ma hater ambiri ,ndipo dziwani kut akadakhala ngat inu akadafo kakalekale.ena anamubifa koma anatopa okha.

 8. kma sunday ku robins kukavuta 1for sorry…2 for grady…3 for nyau munya bola zake zikutheka mot tizisapota kt akutchukitsa malawi chitsiru martse mkono anakumponda

 9. in malawi GD, Fredokiss & Third eye are the best. Koma Martse wachita apazi watenga tsoka nyimbo zako sizizamvekanso pa any malawian radio #mark_my_words

 10. Tay grin is well known inter national raper u cant compare him to peanuts like Gwamba etc.Tay grin has been featured on channel O.wt criteria have u used to come up with nonsense out come.

 11. we the listener are the one who can select the best, osati abakha nokha nokha kumapanga noise ndi za ziii, nonse ndima musician thats all

 12. we the listener are the one who can select the best, osati abakha nokha nokha kumapanga noise ndi za ziii, nonse ndima musician thats all

 13. we the listener are the one who can select the best, osati abakha nokha nokha kumapanga noise ndi za ziii, nonse ndima musician thats all

 14. hahahaha martse thats wasup gwamba,n u not crazy are best raperz …money cant rap ppo do techinacally i gat ur vote

 15. the title of this article is a total joke, whoever wrote this is a total faggot, I mean we all know martse jus hyped this two bcuz they are friends, buh did he mention taygrin??hell no! whoever wrote this is a fan of manganje, gule wamkulu and th like, ain’t kno hiphop at all. that fag martse jus hyped those clowns and you here adding salt to th wound telling us taygrin is shit, bitch pls! we listen to hiphop and we kno whos who so stop crowning these assholes, they irrelevant to th game.

 16. the title of this article is a total joke, whoever wrote this is a total faggot, I mean we all know martse jus hyped this two bcuz they are friends, buh did he mention taygrin??hell no! whoever wrote this is a fan of manganje, gule wamkulu and th like, ain’t kno hiphop at all. that fag martse jus hyped those clowns and you here adding salt to th wound telling us taygrin is shit, bitch pls! we listen to hiphop and we kno whos who so stop crowning these assholes, they irrelevant to th game.

 17. the title of this article is a total joke, whoever wrote this is a total faggot, I mean we all know martse jus hyped this two bcuz they are friends, buh did he mention taygrin??hell no! whoever wrote this is a fan of manganje, gule wamkulu and th like, ain’t kno hiphop at all. that fag martse jus hyped those clowns and you here adding salt to th wound telling us taygrin is shit, bitch pls! we listen to hiphop and we kno whos who so stop crowning these assholes, they irrelevant to th game.

 18. gwamba and crazyG u cant compare ndi #taygrin hahahaha ana muli kutali taygrin anablower internationally kma ena mukuwatchulawo its only here in malawi, Go ku america and ask za Taygrin akakuyankha, u thnk ku america angamuziwe gwamba hahahahaha thats total madnes bwana Martin #matse himself

 19. gwamba and crazyG u cant compare ndi #taygrin hahahaha ana muli kutali taygrin anablower internationally kma ena mukuwatchulawo its only here in malawi, Go ku america and ask za Taygrin akakuyankha, u thnk ku america angamuziwe gwamba hahahahaha thats total madnes bwana Martin #matse himself

 20. gwamba and crazyG u cant compare ndi #taygrin hahahaha ana muli kutali taygrin anablower internationally kma ena mukuwatchulawo its only here in malawi, Go ku america and ask za Taygrin akakuyankha, u thnk ku america angamuziwe gwamba hahahahaha thats total madnes bwana Martin #matse himself

 21. Martse kape!-asaname jelous bas krazy G,amangodalire wena basi!hahahaha maguys muzisata musik and ambri sakutha kusiyanisa pakat pa best rapper nd kutchuka;kkkk suffix,david kalirani,third eye,yung LT macelba hahahhaaa ana mwachepa ntchito kumangoimba zachichewa basi,nzungu akumva bwanj?????? 1 fi sory 2 fi glady 3 fi nyau …….get down-get down!……

 22. Martse Akunena Zoona,ndipo ndikugwilizana naye.#Gwamba akulukulu ndi1 ndipo akamati #Chichewa_anakhoza1 ndizonadi.Adaja amatha Pazifukwa izi 1.Amakuluwikwa /Kuzimbaisa Mau 2.Zifanifani/Kufananisa mau 3.Amasakaniza our local languages in one song.4. Lyming words nde sinkhani In shot I can say #Nsinjiro_zachiyankhulo, munyimbo,Eeeh! amazitsata kwambili.Moti Ukama mvera nyimbo zake,It takes time for you to #think_deep kut umve kuti akuthandauza chani?eg In #Ndiyima_pachulu song he said “Nachikondi kwankazi uyu Yekha sichichoka #chifukwa_gwamba_nkaziyu_anakonda_ngati_njoka”ndinkuluwiko koma ambili samaziwa.meaning kuti “chifukwa Gwamba #Loved (anaconda) ngati njoka,” but instead of using the word “#Loved” he used “#Anaconda” which is the type of snake,#Irespect Gwamba_My_Best_Rappe.Za #aname_anga_KreyzG sindikamba zambiri chifukwa muzaona ngati ndikuwabakira.Kkkkkk .KreyzG naye amatha.

 23. You can be the nations best goal keeper but if you play for a small team somewhere in a village? Tay grin has managed to harness everything that crowns him king.

 24. In no particular order a list of good atist in malawi when we talk about albun music my list has this people

  Tay Grin
  David Kalirani
  Piksy
  GD
  Barry uno
  Fredokiss
  Classic
  Third aye

  DANCEHALL
  Brastol
  Don wagon
  Malinga mafia
  Black jack

  LOCAL RNB
  LuLu
  Skefa Chimoto
  Masco
  Dan Lu
  Onesimus Major Junior

  AZIMAI WA
  I will always respect Blacka more
  Zani Chale
  Sangie
  Sipe

  MALAWI LOCAL MUSIC
  sir Lucias Banda
  KatelOneshing’oma
  Billy Kaunda

 25. Mtumbuka ndasiya kukugaira support mwangotchuka kumene mwayambakale kuzimva?martse dont feel ngat ndiwe dolo chifukwa chot ankolo ako anakuitana kukaimba tharvern yaku USA kkkk

 26. hahahahahahahahaha amatse nd chan!!!!!!!!! mwapenga et. Grin nd wani funxa ma fanz ako akuuzaxo boboh, dnt b deceived! makape ukuwaika pa top-wo africa xiikuwadziwa nkomwe nde ukaphweketse munthu wamkilu yemwe akuimilira malawi ku continent-yi.walingalira bwnj pamenepa

 27. Vuto lako martse ukadya nsima yakwanu ku nkhata~bay ya chinangwa umayankhula zozerezeka , ukufuna chani maka maka ulibe kanthu martse

 28. David Kalilani BBC’s African Best Rapper 2015,BBC African best song 2016…mmmm ma rappers abisala alipo kwabasi,clasic,D1,3rd eye,GD but as far as Malawi is concern Tay grin with his light music is trying his best!But greatest rapper is Jesus Anyambuti David Kalilani ananena kale mu exodus part2.

 29. Its a matter quality music production..gwamba n crazy g are local artist when they cross borders they just normal guys while tygrin is a international star …no rapper can compare him self t grin

 30. Guys r u strangers pa nyasa pano tay grin ndi abwana remmember how he boosted hiphop n mw anawatsegula maso ma yut..stil more pa international amahita he just nid 2 b saluted.

 31. Tay Grin is the one who opened ears and eyes for these stupid kids (Martse,Gwamba …..the list goes on) to start causing noize pollution pa Malawi pano. Then its total marijuana for him to crowned himself az abest rapper.

 32. green musamuyelezeeeeeee ndipo mulekeni ….. ndati musamutchule iye amatha kuimba … iye ndiwandalama … ndiye ndiosamba osat matse manyi ambuzi ngat ameneo … shupit

 33. I think Malawi24 you have just lost your brains……..Martse is not a best rapper and he will never be with his wacky rapping style …..we have best rappers here like third eye , dominant 1,classic , and many more not your martse ……..ASA ka malawi24 ndaka hater kandikhumudwisa

 34. Chifukwa chake macelleb aku mlw mumavala ma sleppaz popita muma opn sho zoona matse Ku fanizana ndi nyau akudichan ka 100 matse nchifukwa mukuyankhula mbwelera zanu # FUCK#

 35. Matse his right tygrin aint the best rapper gwamba ndi crayzie g ndi makapenso check GETTO AMY out you will find the best Rapper in this country

 36. What is hip hop to you? Or what do you want hip hop to be like?…………….. Some people won’t appreciate anythng in lyf. Try becoming a rapper yourself n see de outcomes

 37. Ngakhale gwamba akunenedwayo amapereka ulemu kwa tay grin, anayamba hiphop after drawing an inspiration from tay grin, moti sakanakwanitsa kusiya secular hiphop osayimbako ndi tay grin ndi role model wake, ka crazy g kakunenedwaka mafupa ake sanakhwime mkomwe mu hiphop industry. Dolo amadziwika ndi hit song nanga yake ili kuti? Amadyedwa ndi malceba, mwanache, mpaka dirty flow kkk. Ka martse nde ndikudziwa kuti nyimbo yoti mwano ija ndiyomwe ikumpatsa dziwindi koma imene ija si hophop. Imene ija ndi pasada yamaryhming words kkk. Mwalo moti alimbikire mkumapereka salute kwa madolo ngati tay grin koma basi msanje kaduka miseche mupita nazo kuti agalu inu???

 38. I think before you people start arguing who the best rapper is in Malawi, mudzamvereko “GD” wa Dare devils then start arguing. ….say waaaat say waaaaaaaaat

 39. I think before you people start arguing who the best rapper is in Malawi, mudzamvereko “GD” wa Dare devils then start arguing. ….say waaaat say waaaaaaaaat

 40. Gyz kwa2 kuno umbuli xuzatha bax, zoona munthu wamkulu ngat Grin muzikafanizira ndi ka matse chamba Chan, iye mukuti matseyo waimba zichan zoti azikalimbana ndi Tay Grin? Kufuna kutchuka? Mukamuuze alimbikire mwina azafka pa aGrin, inu mukuwapopa achina matsenu hip-hop mwamba kuixata lit? Chot muziwe Grin ndyemwe anapangixa achinyamata ambir kuisata hip hop, iye uja ma size ake ndi achina phyzo, young k, third eye ndi Ena otero oxat mukut Matse, Gwamba ,Krazy G mmmmmmmm, ndi Ana awa pa hip hop, Grin ndiwa international oxat makape kumaphweketsa , ndipo tianthu timenet sitizafika pa Grin, bore Dem.

 41. Gyz kwa2 kuno umbuli xuzatha bax, zoona munthu wamkulu ngat Grin muzikafanizira ndi ka matse chamba Chan, iye mukuti matseyo waimba zichan zoti azikalimbana ndi Tay Grin? Kufuna kutchuka? Mukamuuze alimbikire mwina azafka pa aGrin, inu mukuwapopa achina matsenu hip-hop mwamba kuixata lit? Chot muziwe Grin ndyemwe anapangixa achinyamata ambir kuisata hip hop, iye uja ma size ake ndi achina phyzo, young k, third eye ndi Ena otero oxat mukut Matse, Gwamba ,Krazy G mmmmmmmm, ndi Ana awa pa hip hop, Grin ndiwa international oxat makape kumaphweketsa , ndipo tianthu timenet sitizafika pa Grin, bore Dem.

 42. You dont know what you are saying Tay grin hes the best rap king and nothing can change that,when people nitced about Gwamba and Martse kids for yesterday stop talking nonsense Grin the best whether you like it OR not

 43. You dont know what you are saying Tay grin hes the best rap king and nothing can change that,when people nitced about Gwamba and Martse kids for yesterday stop talking nonsense Grin the best whether you like it OR not

 44. matse ndikape heve coz sangamanyoze munthu amene wasegula khomo coz anakakhala wina anakanyadira kuti khomo la ma collabo ndi ma artist akunja lapezeka koma pot ndikape osazindikila anzinena choncho

 45. matse ndikape heve coz sangamanyoze munthu amene wasegula khomo coz anakakhala wina anakanyadira kuti khomo la ma collabo ndi ma artist akunja lapezeka koma pot ndikape osazindikila anzinena choncho

 46. matse ndikape heve coz sangamanyoze munthu amene wasegula khomo coz anakakhala wina anakanyadira kuti khomo la ma collabo ndi ma artist akunja lapezeka koma pot ndikape osazindikila anzinena choncho

 47. Gwamba is wack,krayzie g is lame ,Martse is a no show ,the only rappers I respect in Mw are Third eye,Genii blakk,D1,Young Kay,The Daredevils ,Tay grin is now gettin there, to name a few ,

 48. Gwamba is wack,krayzie g is lame ,Martse is a no show ,the only rappers I respect in Mw are Third eye,Genii blakk,D1,Young Kay,The Daredevils ,Tay grin is now gettin there, to name a few ,

 49. Gwamba is wack,krayzie g is lame ,Martse is a no show ,the only rappers I respect in Mw are Third eye,Genii blakk,D1,Young Kay,The Daredevils ,Tay grin is now gettin there, to name a few ,

 50. Worse still oyankhula zimenezoyo akakhale Martse yemwe nyimbo zake ndi eish usandilakwitse….I dont follow hip hop that much but little I know that Tay Grin is gud and I hv several of his songs

 51. Worse still oyankhula zimenezoyo akakhale Martse yemwe nyimbo zake ndi eish usandilakwitse….I dont follow hip hop that much but little I know that Tay Grin is gud and I hv several of his songs

 52. Worse still oyankhula zimenezoyo akakhale Martse yemwe nyimbo zake ndi eish usandilakwitse….I dont follow hip hop that much but little I know that Tay Grin is gud and I hv several of his songs

  1. Libidous Martse Panel Beaten For Skirt Chasing At NRC
   29th March 2016 NRC Correspondent
   Libidous Martse Panel Beaten For Skirt Chasing At NRC

   Local artist, Martin Nkhata popularly known as Martse in the music circles has been beaten by irate Natural Resources Students. Information reaching Malawi Independent indicates that, Martse who once studied at Natural Resources College thought of visiting his former college where he misbehaved by trying to go out with girls who belong to some other guys on the campus. Upon realizing that Marste had closed their line, some guys agreed of panel beating him so that he does not think that being a celebrity means going out with other people’s…Robert Mkwende the guy has issues

  2. Libidous Martse Panel Beaten For Skirt Chasing At NRC
   29th March 2016 NRC Correspondent
   Libidous Martse Panel Beaten For Skirt Chasing At NRC

   Local artist, Martin Nkhata popularly known as Martse in the music circles has been beaten by irate Natural Resources Students. Information reaching Malawi Independent indicates that, Martse who once studied at Natural Resources College thought of visiting his former college where he misbehaved by trying to go out with girls who belong to some other guys on the campus. Upon realizing that Marste had closed their line, some guys agreed of panel beating him so that he does not think that being a celebrity means going out with other people’s…Robert Mkwende the guy has issues

 53. Amatse inuyo track yomwe muna brower nayo outside malawi ndi iti? Popeza Tay Green ake ndye ndi mpweche,mungofuna muwapezese anthu chonena apa eti? Mulibe khanthu inu simunayambe kusambaso

 54. Why can Tay Grin be the best rapper in Malawi??? Mulibemo level yake muno….thats y his songs zimapezeka Ku Channel O..Trace….kuno kulibe size…nanga achina Martse angakaimbe Ku big brother… The guy is just on another level…Zamuwawa anyambite mphuno yake

  1. #Eesha dnt u knw dat yang K,was given total respect kt nd bst rapper by whites in america????????? Hahahhahaa i thnk u r out ov ur knwledge!!try to find out more,kkkkk kumazisata

 55. Martse martin nkhata tamvera izi. I strtd yo lov ur music and followed u as one of the upcoming supa star. Plz lero if u can read ths , uphunzile kukhala odekha komaso if u wanna post somethng to impress two pple jst know tht u will loose fans .# thre z a say; if u wanna make one happy prepare to disappnt alot visa vesa. Taygrin z the best tht much we know and hez one of the gd hip hop rappers kwathu kuno . We hv david.D1.third eye.fredokiss..vice roy.classic.jst mention a few . Samala ndipakamwa pako ndipo if ur looking for haterate soon ur ship z gonna sink believe me. Ndiwe mfana wa bho .whre z the martse odekha timamudIwa uja . Iz it miracle money tht hv changed u?. U hv disappointed us

 56. Kodi Amatse mudayamba kuyimba kuti muzipikisana ndiazanu? Kapena kusangalasa anthu? Mutichitisa manyazitu khalani ndiwulemu ngati munthu ochokera ku Mangoni

 57. Zoonadi yamzy Tay grin it’s another lever man.amalawi kupusa ndi sanje ndiye amadziwa iwo basi.paliso woyimba apa kuposa Tay grin?kkkkkkkk

 58. Personally…Slessor is my favorite… but Tay is not bad…it’s all just a matter of opinion… clearly Martse has his own..koma to say kuti gwamba is the best rapper nde ndi bull-crap…krazie G ain’t that bad either but he ain’t the best too…**fact **

 59. At last I would lk to congratulate pple who involve in voting so I! Justice Isaac wth the power Malawi music I would lk to announce dat Mr nyau king ty grin z the best rapper in Malawi &gwalad com second according to ur vote

 60. Ndie kukhala M’malawiko kumeneko nsanje basi!!!. #Taygrin is duin it big amatipanga represent ndi abwana ; zawo zinayera see on #Tracechanel the #Chipapa track. Just work hard nanunso mumatha its true. #learntoappreciate

 61. Ndawelenga ma comment onse ndaona kuti Martse ndi mtumbuka ndiye tidziwila atumbuka muja town muno anabwela mochedwa + atumbuka kupepela.

 62. Tay Grin ndi dolo basi..martes mungatani…. Nanga poti gwamba wakoyo anapangapo collaboration ndi Grin. Oyimba apa Malawi beef basi

 63. guys but Martse ddnt compared tay grin wt gwamba and kraz g..he just said krazy g n gwamba are best rapper according to him ..like to me its CLASSIK n THIRD EYE

 64. In general Nyasaland got skill kma zomaikana pa scale nde zokanika..why is he tryn to be like an educated savage…kuli achna Genii blak,3rd eye,D1,David kalilan,..just to mention a few…Aliyense amatha chfukwa nose smunga ymbe style imodz..

 65. Guys Let Me Tell You One Thing,all Those Niggars Are Doing Well,but When We Talk About Malawian Hip Hop Tay Grin Is A Best Lapper.Anayamba Nkale Zinthunzi,he Has A Potential.Looking On His Collabolations With International Muscians, It Just Shows That He Is Doing Alot On Music Industry.When You Watch His Videos He Focusing Much On Our Culture.For Example Gule Wankulu,amajambulitsila Ku Mudzi,as Well As Kunyanja Which Also Attracts Tourism In Malawi.Osat Kumapita Mma Town Ku Kajambulitsa Nyimbo Akut Kufuna Kufanana Ndi ;50 Cent,lil Wayne, Bird Man.We Are Too Far To Reach That Point.Tay Grin Is Doing A Lot In Doing Our Local Hip Hop.We Cant Much Our Hip Hop With Ameran Hip Hop Style.Martse,gwamba You Must Learn Something To That Guy Osat Kumadzipopa Cause You Are On The Way To Perfom Great.You Are Not Yet A Lil Lapper Boy

 66. Tay grn nde yemwe yaiika malawi pa map #matse ndikandan kuimba kwake kut kot pakana kumathoka zakabutula kumenyedwa kuja kunakupengensa yet nde azako ukwachulawo HpHP yake iti yot pa kukhal best manyi enieni kumalawi nde kona nachokako buuuuu zopusaaaaa

 67. Tay grin oloko ine samandiwaza, ndipo hip~ hop yake yokomera kumavina tizidole nanga chi nyunyu~nyunyu ndiye zichiyani kkkkkkkkk kunganva kt local hiphop et kkkkkkkkkk

 68. to cherk on ua phone, u’ll findout dat u hv mo songz ov gwamba and martse dan dat ua xo calld tay grin… iznt dat funyy????? #ThirdEyeIsTheBest

 69. KODI DZINA LIMENELI LA MARTSE TANGOLIMVA POSACHEDWAPA PAMENE ANAMENYEDWA MUMSIKA NDI OYIMBA WINA CHIFUKWA CHOSALIPIRA MOWA WA KACHASU WOMWE ANALEPHERA KULIPIRA ATAMWA KU BANGWE.KOMANSO DZINA LAKE LIMAMVEKA NGATI LA MUNTHU WOTSILIKA NYUMBA CHIFUKWA LIMAMVEKA NGATI LA SING’ANGA.ZOTI NDI WOYIMBA MUKUDZIWA NDI INU IFE TIMANGOTI NDI DOKOTALA WA ZITSAMBA NDI PAMENE TIMAMVA KUTI AMAYENDA NDI KAGITALA KAKE KUMAIMBIRA NYIMBO AZIMAYI NKUMAMPATSA UFA.

 70. Best Ril Hiphop Starz In MW R,First Third Eye,Dare Devils,Fredokiss, Dont 4gt Wankulu JB Not Gwamba O Crazy G.Who Dis Shit ,I Dont Like U Martse 100%

 71. china phones + free internet,,its where i can put ma blame,,,anthu ambr akukambapo nkhan zomwe sadayenera kukambapo,,ndpo sakudziwapo kanthu,,,kma eish!! pakufunika #civic_education apa,, sitiziwa zambridi amalaw kmano access to internet its where the problem emerges,, i rest my case sir

 72. kulitu ma upcoming rapperz ku Zomba osati mbwelera zomwe mukunenazo……. Bwelani ku Zomba muzaziwonera nokha a Matse,,,,,, vuto lakusayenda mma show,,,,,, panopa akutiimilira ndi Ty Green on top bas Winning.Com

 73. Tay Grin is the best music motivator, he inspires and gives ambition to youngings, every body wants to a successful person just like him….. Not like a faggot celeb who was humiliated at his own college campus because of nyama yambuzi

 74. TAY GRIN NDI MACHINE BABA AMATIIMILIRA MAKA POSAIWA GULE wamkulupo pamene ndinaziwa kuti akulu amanyadira ponkhala malawi keep it up osasiya..,… osatopa

  1. koma akuyipanga play pa Trace..nanga amene mukuti amathawo nyimbo zawo munayamba mwaziwonapo pa trace ??..Chipapa olo uziti ndi mbola koma ili pa trace..idiots

  2. Inuyo kaya u like him or not but… tay grin he knows how to rap osamaphwekesa zanthu akamachita bwino koma kumuyamikira

 75. its not hidden fact that Tay Grin is not the ‘best’ rapper in Malawi. but saying Gwamba is. then that’s just overrated. trying picking amongst Young Kay David Kalilani Dominant 1 Third eye. we can agree to disagree.

 76. No hard feelings. Taygrin behaves more of a DJ. Most of his songs are not original compositions. I hope someone has observed what I see. Martsee is relatively new on the seen, with remarkably one hit song. Nothing else to talk about.

  The Gwamba guys , on the other hand, have original songs. What they do lack is raising the bar for themselves. They haven’t marketed themselves that much beyond our boundaries.

  For me, Gwamba is comparatively better than Grin.

  1. Man…that’s crazy..none of these cats is original…none of em is unique..so basically none of these guys is a rapper..they all do hip hop.. which is not rap at all…so why bother draw comparison???

  2. Well, i might not be right with the facts my comparison, Innocent. However, I do listen and follow both local and international music. I love music I should say. Hence my audacity to contribute to the debate. The expression in my contribution is how I see things on the ground. Others might see differently…and I have much respect for that.

 77. I respect hs views & i hv to say that he is a rapper so he should concentrate on sharpening hs skills nt telling us who to luv, hate or overate as the best, keep on being a rapper broh & we wl b the better judges, respect to all the rappers

 78. That’s his opinion. Stop trying to blow things out of proportion. Y’all need a reality check! if he thinks Gwamba and Krazie are the best as compared to Tay then so be it. Clearly the writer does not understand the notion of ‘Free World’. Lets not forget that we are all different and we also have different opinions. Why do u want to start beef between these two guys? GROW UP!!!!

 79. that’s why I love reggae music. no hatred, no negativy. it’s only peace and unity. freedom and equal rights for all. reggae loving forever. peace!!!

 80. Grin has been in hip hop game since wayback, Gwamba wabwera liti kuno? Kodi Martse ndi ndani? Who the fuck is Krayzie G?…. We can talk hip hop without mentioning these three idiots….

 81. Amalawi simutha kutukurana koma majerasi ba mmalawi muno muribe oyimba ngati nyau king oro aja mmati sir aja sangafikepo oro mphasha gamoto oro mametedwe oro kadyedwe grin ndi namba one mmalawi muno inuyo level yanu ndichina chibade rusiyasi jeo gwaradi kapena mbenjere uja amati tiye ku church

 82. Amalawi simutha kutukurana koma majerasi ba mmalawi muno muribe oyimba ngati nyau king oro aja mmati sir aja sangafikepo oro mphasha gamoto oro mametedwe oro kadyedwe grin ndi namba one mmalawi muno inuyo level yanu ndichina chibade rusiyasi jeo gwaradi kapena mbenjere uja amati tiye ku church

 83. Mpanvu yakusazitsata,tiri ndi ma rapperz osati mbwerela mukunenazo..Gwambaaaa hahahaa! Martseee kkkkk koma inuuu! They ain’t complete rapperz,they still relay on others to do hooks for them,listen to Third eye and David Kalirani js to mention afew..muzadziwa wat rap iz…mwina simunva kuti akuti chani wen they r doin it.

 84. Though i should respect the reapective choices for Taygrin, Gwamba,Crazy G and all the other urban music artists of course for various reasons but my take on this one is that Malawi has only one true ambassodor in hiphop and thats none other than THIRD EYE.Listen to his music carefully without a biased stand you will really accept the fact that this guy could make Malawi go far beyond in as far as hiphop is concerned. He can sing in very good english,very well articulated facts with the songs and instrumentation well balanced. Otherd are in hiphop because of money from their parents,others just to put a name and gain fame,what they sing nobady knows thats why their songs only enjoy a atwo week airplay,lucky they bribe Djs.

  1. Slob Slob, i really respect David Kalilani, he is another guy with his own style of gospel hiphop,just like the way Wisdom Chitedze was. The only thing may be could be his beef with Bushiri if it is true,that some of us may start saying,look,he is a gentle man but now he has started crossing the line but any way he is really good.

 85. I’m a Malawian.aged 26 but I’ve never heard such a name (mwati martse) nyamata kapena nsikana…amakhala kuti.amatani..tanenani…uncle Grins own one

 86. apparently.. aliyense ali ndi rapper wake who he considers as the best… but what i know is Taygrin is and remains to be the only heavy weight, internationally recognyzed malawian rapper so far.. I hav never lyked his lyrics tho coz they never makes anysense to me but he knows how to maintain his game.

 87. Martse must be out of his god damn mind,,,,,,,,can you compare Grin with crazie G or Gwamba???,,,,,like seriously? or eniakewo akhoza kukanatu zimenez,,,,mwina ndichifukwachake zimakuvuta2 martse umadziika pa #zero pa gulu la #Makape

 88. Nenani zoti ma rapper enawo amatha,koma osati zoti ndi a Phyzix omwe amatha,,,bola muzindiuza Dare Devils kapena Classic ndiziwa kut mumayisata Hip Hop… #peace

 89. mxiew zausiru eti ndimadana ndizoposatu am not jocking…Am serious osapanga zanu bwanji mukulimbana ndikunyoza ndichifukwa chake ku malawi kuno kuimba sikupita patsogoro nsanje too much

 90. Kodi nanu amatse mwaziziwa liti zoyimbayimbazi kuti muzikalimbana ndimafumu njila yongofuna kutchuka chani ndiye kuti uziwe kuti grin ndi abwana sakuyankha ngakhale pang’ono msete zakozo forsake!

 91. Zambia is in the building….. Tay grin is doing great in Zambia. He’s the only rapper i know from malawi who got content and hiphop flavor. they say they balling koma zigoli ni zero… TayGrin is hard. #Chipapapa #2by2

  1. He is a multi-millionaire, over K300M so what do you expect? He markets himself and do songs with stars but he is wack. He just sucks on Mic and thus why DJ Lomwe beefed him too hard that he had no guts to reply but say he has no beef with anyone only later to have an abstract beef aiming at Lomwe. TayGrin is wack!

  2. I respect yr opinion man but lets face fact can u market what pipo hate?. Can pipo buy into ur product if u are whack?? I don’t think so. If he’s wack as you say why did he win the BEFFTA in UK for Africa??. TayGrin is selling Malawi to the world and u call him wack?!..TayGrin did a song with Zambia’s bigest and best rapper Slapdee in 2009 but still the song is a massive hit.. TayGrin got no levels. And for a thought ask yrself why Nas was beefing JayZ…. #Chipapapa

  3. They just want to bring grin down, but you idiots won’t make it.. If he is wack why is he a top selling artist in Malawi?. which hip hop artist can compared to Tay grin.. munazolowera nyimbo zo bifana that’s why yo so called favourite rappers ain’t go no way.. to the hell with yo local rappers.. it’s not about maso anga anayamba mwano but #Chipapa in high definition

  4. Still am a fan of tay grin other people just hate him because his rich but when we talk about music always i sailute him big up man taygrin

  5. Still am a fan of tay grin other people just hate him because his rich but when we talk about music always i sailute him big up man taygrin

  6. #AbelSingano this aint about XYZ or General kanene. We are talking about Malawian music here.. are u just an illiterate that you couldn’t read the subject at hand. Plus General Kanene was jailed for raping a minor… #TayGrin is ever on point like a decimal. #HatersTakeABow

  7. kakakaka taygrin? realy surprizd hw u o would say tay grin raps betten than the rest rapperz in malawi, u mst be disaranged sum hw this tay grin is out there crackin bcz of his cashgatin cheddar without that he wouldnt be at this exposure of platform.we got lot x factor rapper jst to name we got thrd eye,clasik and any other best.they r not recognisd very far cuz of money.we gvs less dah fck hw tangible/skiled tay grin is when comes to blending and fusement of other legends traks.

  8. Do you know TayGrin pays the DJs to play his music? I even revealed that last year on my wall. For instance that remix he did with Brick n’ Lace he paid the radio 2 DJs K10 000.00. The song had more than enough airplay. I can tell you a lot what DJ’s do and what an artist has to do to be heard. Just like Hazel Liyaya, she has money so she is getting played. #Truth_Reality

  9. Do you know TayGrin pays the DJs to play his music? I even revealed that last year on my wall. For instance that remix he did with Brick n’ Lace he paid the radio 2 DJs K10 000.00. The song had more than enough airplay. I can tell you a lot what DJ’s do and what an artist has to do to be heard. Just like Hazel Liyaya, she has money so she is getting played. #Truth_Reality

  10. #Ralph are u sure TayGrin Zambian DJs, Namibian DJs, Nigerian DJs and TraceTv video chart management just to be rated the best in Malawi??.. I dont think so. Even if you had to bribe the whole African DJs if your music is whack people cant appreciate it.. Good music is good music no two ways about it. Are u telling me Skeffa Chimoto bribed the south African and Zambian DJs to be appreciated as he is in these countries??.. I don’t think so.
   Look at our very own Zambian Musician JK who did 2 songs wit R.Kelly just to gain recognition on the world stage but did he?, Was he recognized??, no he wasn’t. But R.Kelly is a renowned world figure a music icon but why didn’t Jk songs gain massive airplay on the African continent??. Because the songs were whack they lacked credibility, creativity and attraction despite collaborating with R.Kelly…
   So give credit to TayGrin for putting Malawi on the map. Did he bribe the BEFFTA committee for him to win?? No mahn. Give juice to this guy coz he’s got game..

 92. Ai guys tisanamizanepo apa pa za woimba pa malawi womwe ama rapper kuti awa kapena awo/anja amatha ku rapper, Ali yense munthu amakhala ndiwomukonda wake yemwe amamubva bwino mumtima…. Anga manganizo ndiakuti mwina pangokhala mpikisano wa ma rapperz one by one ndiye anthu apange ma vote kuti King ndindani yemwe wapondele amzake. Enawo mwina amawoneka kuitha kamba kukuphatikizana wina ailowe winanso ailowe yomwe yomweyo.

 93. A Matse muzikangolimbana ndi achina Mafo kapen Gibo ndye ma levo ako!Iwe siomusasa 3rd eye jaket atagwla mic!Wayamba lit kuimba iwe?kanyimbo kake kati?Anthu ngat inu ndi amene mukuononga hip hop industry!

 94. kulimbana ndi tay grin imeneyo ndi minyama2 kk anzanu anayesesa kt amugwese zinakanika ndi wat more makaphula mazira ngat inu #martse #gwamba #crazy g mukungotaya nthawi yanu. limbklani tizaoneleko nyimbo zanuzo pa trace makapenu nzanu #taygrin dairy tikumuonela pa trace so whoz the best pamenepo hahhahahahahahaha nonsense

 95. Apart from from rapping grin is big man i prove it myself nthawi ina yake tinamugwirila job,tikakamba zo rappers dictator ali boo plus junior c,level ina basi akupanga zomwe timachita chaka chatha panopa level ina level ina level,enawa bvubwa

 96. if u respect rappers like third eye u stupid because they doit in an American way but Tay does it malawian thats why he number 1…why try to be like an American rapper aint that stupid really

 97. grin is best salary ya m’dala ya martse ndiyomwe grin amagulira ma tisue a siku limoz, gwamba ndy ndaninxo gwalad atha kugwesa zimenezo

 98. Matseyo ndi kape pamodzi ndi maflambo anzake osatha kuimbawo oti olo pa Gwaladi sangamake //madolo apa Nyasa ndi Fredokiss,David Kalirani,Pop Dogg etc osati Mbule akuzipopazo Alaaaaaaah

 99. Ndilibe nazo khii or mukuti anaimba ndi 2baba otchuka,or ndiyemwe apangisa our nation kufika pa map,sindikuwerenga wat i knw samatha mwa iye luso mulibe amachita kuzikakamiza mix cash yamakolo basi winawe wagundika kumupopa,zachamba satha satha basi finish story

 100. Chimene ukuyenera kuchita iwe so called ‘martse’. Jst go n ask Tygrin njira yoti azikuikanso pa trance tv or pa channel O not kunyoza de ‘KING’.

 101. chipapapa papa >martsetsetse tsetse{ty grin we respect u coz u take our malawian music to the intelnational level{aaa malawi music}

 102. Not the best rapper but the most loved rap artists currently…..even most of the kids r his witness…..my three year old cousin loves the chipapapa song….

 103. Duin lyk dnt kno musicianz, Tay Grin iz nyau king wea az Martse Cosoma, they r different. Jst lyk a Chicken and a duck, vey r really different.

 104. kkkkk martse kkkk ndimangoseka wina atapanga upload pic ya martse a akuumbuzidwa and ali mbuu kutuwa wina anakomenta kuti “martse kutuwa ngati amamupala ndi mpeni”

 105. Gamba wa suit ndi nda? Kodi banker wotchuka ndi nda? Ndimadukulitsa mabeib zantchito,, ndine mfana wachikoka ngati ginito hahaha phyzo apa basi ndi mzake mwanache osat zachizungu zanuzo achina D1 anuwo ziphwisi mpake akanali pakhomo pa masten munthu nkulukulu

 106. Martse ndi kape or xool sanapite wayeneraso kukhala mulimi wa fodya or msozi ,Munthu osasamba ngati martse azilimbana ndi madolo ngati nyau king

 107. My comment goes straight to Tay grin>u r the best komanso don’t forget kuti munthu ukamakhala ndi ma haters ambiri just know kuti u r doing more than they expected (za jealous ku mpanje kuno tinazolowera)

 108. Akungofuna kutchuka mwanawang’Ono ameneyo malo molimbikila mbaliyake akupanga zawena muuzeni kuti ndikape ameneyo ndipo nyimbo zake zili pà région leval sanafike nkomwe pà national level ndiye nkumalimbana ndi munthu oti ali pà internacional leval haaaaaaa Grin yo zake zinayela kalekale kamantse ko kakulila ndi nkodzo wake omwe uliumwana shame on mantse futseck

 109. David kalirani ndi deal. ena onsewo m’bwerera zokhazokha. CHIPAPAPA nde chani? za pansi pa…………… ei papa game yalakwa apapa.

 110. anthu okhao amene mutu wao sugwira bwino ntchito ndi amene amatero

 111. David Kalilani ndikatundu..Third Eye ndi mthutha…D1 ndi makina.Classick ndi Best..Viceroy ndi nkhani zina..Gd Ndi Massive….Madolo awawa ndi nkhani zina osati enawa

 112. very true ……….tay grin wangokhala ndi dollar luso alibe…….akanakhala kuti makolo ake ali ngati a enafe bwenzi ameneyu asanadziwike

 113. Martse siutha iwee usalimbane ndi nyau king Tai Grin amakwana,iwe uzingokhala choncho ndi chidazicho,mxm kape wachabechabe iwe

 114. Antu umbuli understand the story martse was asked his views about the best rappers and he chose those guiz,but just cz these reporters wants to lure u the start the story as if martse said taygrin is not the best…here comes ignorant malawians mpkana kunena dad wa martse zausilu understand the story

 115. A martse mwayamba kuzipopatu Mpaka kupanga create debate nkumati Tay grin z nt a bst rapper kkkkkk

 116. kwakwakwa..so srry for you martse and who are u compare to tay grin… as I can see the cap itself haaa fake bru and u rocking in fake brands haaa even too far to compare wit ME ..tay grin iz a real rapper dude…haaaha interesting I even know u today hahaaaa

 117. Who is this ugly dude called M**y? Th only tym i heard of this sh*t name is when i tuned in to a certain Malawian Radio Station & i was just eager 2 know who this creature, flu-obsessed & desperate rapper to be is all about? Ok, he is tryna go in2 feud wth th only rapper i (we) kno from Lagos? lol!

 118. martse-Ndi wa jelous.pajatu anatchuka ndi nyimbo yoti “mwano” poti ndi “wamwano” akuchitabe “mwano” maso ake ndi “amwano” akuyankhula “mwano” zochitika zake ndi “zamwano” mwano=jelasi + ufiti.martse,a badman

 119. Kodi Matse umanziwanso kuti Taygrin ndi bwemba weniweni eti kkkkkkkkkk aaaaaaa alibe luso Taygrin ndi kape ndalama ndizake zimenezo Matse wanena ngamo

 120. A Matse Ndiwe Kape Kuimba Wayamba Liti Moti Mulimbikire Kuti Nanu Mufikepo Pa Tay Grin Wayamba Mwano Ngati Nyimbo Imene Unaimba Ya Mwano Basi Sindizaveraso Nyimbo Zako . Kodi Nyimbo Zako Akuziziwa Ku Uk Ukhala Pomwepo Tay Grin Akupita Pasogoro Ndiye Koma Ukuona Bwanji Chipapapa Mene Yagwilira Sewu Zkozo Tizingombena Jerasi Ngati Mkango Unakhala Bwanji Moti Muzifusa Kuti Ungaimbe Bwanji Ukuyakhura Mwano Tay Grin Sungafanane Naye Wava Matse Matse Chani

  1. NOSENU NDINU MAKAPE KUPHATIKIZAPO MATSE WANUYO MUKUONEKA NGATI AZELU KOMA MULI MAZOBA NGATI MATSE WANUYO ANA INU MUKUZIWAPO CHANI TALIMBIKIRA SCHOOL KOLOMO ANU ALI MOYONI

 121. oh shame Tay Grin He’s the head of Malawi and achina matse anuo ndimafana kwambiri tay grin ndiotchuka kuambila kale no one can compete with him kwama rapper onse akubwela pambuo pake no matter what olo atakaimba kwameleca dziko limakhara ndinduna yoyamba and if i may see amalawi you have too much jealous shaaaaa chonde tasinthani please Malawi sitchukatu coz of mtudzi mumapangao Guy’s let’s respect Tay Grin.

 122. Krayzie G amatha koma ndmfana ofooka pamene Gwamba amalimbikira koma analowa mbola, Tay grin mmmm mmhu amatiika pa map pot anthu akutero

 123. Onse akutchulidwawa sangafike pa Phyzix. Bola mukananena za Third Eye, Daredevils. Enawa amangotchedwa ma rappers just because they rhyme no matter their lyrics don’t make sense. Komanso Tag Grin amaoneka kuti amachita zokakamiza, his rapping style lack flavor.

  1. Phyzix is one of the wackest rappers in Malawi dawg ,he has no creativity in his flow ,no rhymes ,the guy sucks big tym……im not hatin koma its the truth ,do a research

  2. Phyzix is one of the wackest rappers in Malawi dawg ,he has no creativity in his flow ,no rhymes ,the guy sucks big tym……im not hatin koma its the truth ,do a research

  3. Phyzix is one of the wackest rappers in Malawi dawg ,he has no creativity in his flow ,no rhymes ,the guy sucks big tym……im not hatin koma its the truth ,do a research

  4. Tay grin amazikakamiza ngati 50 cent amazikakamizila. komano amatha chifukwa akafuna kupanga chinthu amatsimikizadi zonse zimakhala perfect .size yake kunoko kulibe guys .Muntha kuzayimba bwino koma sumuzafikapop chifukwa zoyenelela mulibe

 124. Who is MARTSE ?.what does he do for a living?. I just open the link and read, I also see this guy called martse who is saying that Tay grin is not a rapper. This martse sakuwonekaso ngati musician.ati wavala timagalasi kaya ndichani china kaya koma akulimbana ndi munthu oti ali times 10 kwa iyeyo. kufuna attention basi. olo bambo ake a martse pa Tay grin sangafike.. Grin is the only hip hop artist who put Malawi on a map. wina asazinamize kuti ndi dolo than Tay grin..Martse nde ungozivuta chifukwa olo ma punchlines sumatha kape iwe.. sanje basi

  1. Martse olo alibe chilichonse koma nyimbo zake ndimazikonda Tay grin mmmmm ndimangomva olo kupanga downlord ndimamvera kamozi yandikwana.Martse ndi deal kkkkk

  2. Stupid news frm malawi 24 mwapanga post zaboza ife taona post yeniyeni inayo ndiyanu yaboza matse was lyk as long as asay kranzie g and gwamba r de best rapper he mean kwa iyeyo he dn’t say ee taygrin or any one apart frm those two guyz nde isee no any reason to put ablame on matse ife timafila makawa one day we will post dat makawa is de best eva zidzakhala kwa ineyo osati de whole nation paja zokonda kusiyana

  3. Ine ndunena zonse, dollar plus talent. akanakhala kuti martse yo amatha why nyimbo zake olo pa channel sakuwonetsa.. Ana anzake achina YCEE ayamba pompano kuyimba koma nyimbo zawo pa channel O and Trace akumayika always.. Nde munthu osasamba ngati martse azilimbana ndi Tay grin oti akumapangidwa ma nominated ku UK AWARDS.. Tay grin wapezaso dollar zambiri because of his music career.. Kodi Mesa martse so ali nda bale ake kunja ochita bwino, nanga bwanji iyeyo alibe dollar kuti azilipira ma international artist for collaboration,, ngati mukukamba zoti grin has money not talented.martse also belong to rich family but he is not popular, which means he is not talented..Ndiposo samaonekaso ngati artist.. akuyimba nyimbo za kachasu, ati Mwano kaya Chani Chani uko, pin ya blackberry. angachuke ndizimenezo?????.. he is just wasting his time coz grin is not his type.

  4. anthu ena simumazitsata in a song muzikhala samthin yo communicating to the world osamangopanga za soulja boy apa. Anyambut ndi more talks real life issues

  5. kkkkk u cant compare ycee 2 martse aixe, they hv mo acces to thoz channelz. wat u r duin itx lyk comparing jayz to diamond,, do they match??????? Tay grin iznt the best rapper in Malawi, he jst knw hw 2 spead hiz music widely…

  6. Martse mwangozitukanixapotu apa, tay grin is not ur type ndipo ulikutali kwambir anyway limbikiran bwin muzafike pomwe grin wafikapa always dream in colour.

  7. A Martse akufuna potchukirapo.Anyway limbikirani mwina muzafika pa Tay Grin. Koma zoimba zanu zimaoneka zachibwanabwana simungafike pa international level bola Gwamba amayeselako pang’ono. Tay Grin alibe nzake mmalawi muno

  8. Okmalumkoolkat Buliana osati nyombo zaku aBAR koma tikutiku munthu ukamanvera nyimbo nawe nkuchita kunva bwino kuti munthu akuyimba apa ,nanga abale zoona munthu kupitq kushow kumakanvera atiii 2 by 2 culture aaaaaaaaa zoona ndipo olo itakhala yaulere nsingataye nthaw kukaonera aaaaaaaaaaaaa

  9. tay grin anatchuka coz ali ndi dollar and he has all support from his parents coz nawo ali ndi dollar david amatha martse amatha koma anthuwa angosiyana financial status luso ndi ndalama ndi zosiyana koma pena zimayendera limodzi

  10. Vuto a Malawi ndi sanje.. nanga skelewu ya Davido ili ndi meaning?.. koma Davido anawina two times African of year in MAMA’S AWARD..Martse still have a long way, bolaso Gwamba ama rapper bho. martse olo voice yabwino alibe. akamayimba ngati akungokamba ndakatulo.. 2 by 2 anamenya bho nkona inachuka countrywide .which track yomwe anayimba martse ingapangidwe compared to 2 by 2 ??.mwapinduranji,mwano,grace chinga zonse ndi mbola and they’re is equal to Gwamba feat Nesnes _bola kusache.

 125. Hahahaha watching chipapapa on channel 0(international) pomwe mwano n zikhala better(local) on times tv kkkk go tay grin go chipapapa nsanje siumuna mkani anakumenya chifukwa cha kachasu

 126. amartin nkhata yu a jealous ….tay grin kumbalilake amakwanisa ….& tu mi its abest rapper ……nsanje amalawi dats y muzikamba zanzanu akupita patali big up

 127. Vuto la ana osasamba mukamwa kachasu mwa senti..mmayamba kuona zinthu mwa opposite ukhale munthu oti mutu wako umagwira ukanakhala Martse …