Sleeping George Chaponda breaks the internet

Advertisement
Albinos Malawi

He may perhaps not have slept well enough in preparation for the opening of the parliament on Friday but newly appointed leader of the House, George Chaponda has seen his images which show him in deep slumber when President Peter Mutharika was making the State of the Nation address in parliament yesterday hit the social media as a storm.

The images have gone viral on the social media and a greater number of people argue sleeping meant that he was bored by Mutharika’s speech.

George Chaponda.
George Chaponda spares himself some sleep when Mutharika addressed the house.

While most of the people say Mutharika’s speech was impressive and that the Malawi leader managed to outline his government’s plan on every itching issue, Chaponda and others may not share the same feeling if the slumber they fell into before they met the wrath of cameras is anything we could take seriously anyway.

One of the eye catching comments wonder why it would be interesting that Chaponda was sleeping in parliament when sleeping is normal.

Edna Abiti Kadango wrote ‘To me its not news!people sleep even in churches when the pastor is preaching the word of God!why not in parliament?

However some people who have been commenting on various Facebook pages say Chaponda did not portray a good gesture by sleeping while taking into consideration the fact that he has just been appointed the leader of the house and that his Agriculture Ministry was one of the sectors Mutharika had given a special focus on in his address.

Ausman Nyirongo wrote ”Just imagine. Opening the budget meeting then someone is busy asleep.it shows that you are not interested about the speech of the president. Ok don’t hesitate fire them they are too old.”

A debate on sleeping on duty has been ignited on the social media with people having miscellaneous defences to their stands on the matter.

In his presentation at the opening of the budget sessions, Mutharika talked against the social ills including the trendy attacks on people with albinism and maintains his government will not relent to deal with the perpetrators.

Advertisement

396 Comments

 1. He is sleeping in parliament yet he says Malawians should work hard to develop the country.

 2. Abele,ndiye kuti parliament ndiyolemekezeka kwambili kuposa ku church.?chifukwa akulu akulu enanu mwagundika ndi mbalume mukapita kopephera simulephela kugona.A malawi 24 mudza lembenso anthu church.

 3. OUR COUNTRY HAS BEEN THROWN TO THE DOGS. PEOPLE HAVE TO SHAME TO THE EXTEND OF SLEEPING IN PARLIAMENT, MEANING WHATEVER IS BEING DELIBERATED IS NOT IMPORTANT TO HIM. HOW THEN DOES ONE CONTRIBUTE IN THE DELIBERATIONS, IF I MAY ASK. I REALLY DO NOT KNOW WHAT WILL BECOME OF THIS COUNTRY TEN YEARS FROM NOW. GOD HAVE MERCY ON OUR COUNTRY.

 4. so wats wrong?its normal to sleep y others sleep in church while others sleep in other meeting after given 500000 for 2 days training so wat about parliament or any constitution about this? plz pple tiziona zolemba and post

 5. akagonagona mapeto ake akulandila allowance, munthuyo is gone already koma mukumuika pa mpando ndimenezi akugona Malo oti pali anthu ambiriri akukambilana zomwe akumbila iye sakumva, choncho tingapite pasogolo?,

 6. ndiye abwanawo akuti chiyani iwo akuyakhula wantchito akugona.Sichina ayi munthuyo akumugwiritsa ntchito kwa mbiri ndiye anali atatopa

 7. Inu amene mumanena kuti achoke ,mukudziwa kuti chisime chimaoneka chakuya chikaphwa. kuti asiye mpando zinthu siziyenda bwino. Apresident powasankha awadalira.choti mudziwe ntchito imatopesa. Achaponda More fire.

 8. Zomvetsa chisoni kuti lero a Malawi ambiri tikusangala tikaona mnzathu zikamuvuta. Kodi ndichachilendo kuona munthu akuwozera kapena kugona pamene wina akuyankhula. Kalanga ine dziko langa likupita kuti? Ambuye ztithandize ndithu.

 9. Remember he is a human being just like u he olso get tyres just like u he olso need rest just like u he can olso feel hungly just like u so I see no reason why u pole making noise if u r good at toking shit write ur own novel and make money and celebrate with ur wife rather than tolling shit stop it he is my mentor I admire him he is abig msn

 10. Being the former foreign affairs minister, he has been representing Malawi in a number of international forums. No wonder Malawi is not benefitting much from such meetings. Bwanawa amkangogonako, Kkkkkkk.

 11. Vuto losankha anthu ogonja kale ndilimeneli,,why can he sleep when important issues are being tackled by the president ,it shows he is no serious at all,,mpaka kumalota ndithu #”shame”

 12. qkuyenera kugona kumene.Mwina usiku onse iyeyo anali busy kulemba speach ya president yomwe amanena mu parliamentmo.ndiye mumafuna kut akhalenso busy kumvetsela zot walemba ndiye yemwe kapena amvetsere zot akuzidziwa kale?

 13. wina aliyense amagona sizitengela udindo kapena nzeru.. Imenei sinkhani yoti ndikumatha nayo nthawi.. Kodi inu mutatopa simungagone? Aliense akatopa amagona basi…

 14. Oooh i cry for my beautiful Malawi eish;( really sleeping in parliament is this for real? Ooh my God so do we think this people can lead Malawi in right way? Nowander Malawi is the poorest country in the world, how can someone sleep on duty this is shameful that’s why we so called sleeping people, can someone come nd take over this country plz Army what ar u down take over this country plz we have no direction we have no leader we have no future in this country, bt by the end of month he wil get paid our money whts the f**k!

 15. My psychic readings focus on positive thinking & positive change. It may assist in bringing clarity to a confusing situation, help you prepare for the future in a more focused way and may empower you with positive potential. If you are seeking spiritual guidance with your relationship, marriage, love, family, career, money, health matters, or life’s daily issues, my insightful accurate psychic reading will help you answer the questions that weigh heavily on your mind. I would love to assist you with making the best decisions for your Future. No matter where you live I can help you.Call +27738951830 MUNIL SALEH, I do Whats-App, Face book/munilsaleh, Phone and personal readings.

 16. Ngati Ambuyeyesu anagona mu chombo pa nyanja mafunde akubwata kooopsa, ndiye mukuti mu Parliament (mfwe -mfwe -mfwe -mfwe) with ur bad coments, these people work tirelessly, Jesus was also tired too after his teaching

  1. Luckly, Jesus wasn’t sleeping it was the beginning of his lesson on his syllabus and its conclusion was Why are u afraid off when son of God is on ur midst. But to this case, The Chaponda is tired we’ve been hearing of him since 1994. He must pave way for the youth to take over who can fail to perform

 17. Ngati Sagona usiku amapita kuti?Amakachita chiani?Its better to sleep in his car not such a place.Anthu Omwewa atakupeza ukugona kuntchito kwako ili ya m’boma akhoza kukuchotsa ntchito.Utakhala wogulitsa malonda akhoza kugula wina.Utakhala Mlimi siungakolole.utakhala kuti ukulemba mayeso ukhoza kulakwa.car accidents are sometimes caused by dozing while driving.Uka Magona malo osayenera amathanso kukubera zinthu ngati ndalama,phone therefore awawa ndiye kuti sanamve zimene zimakambidwa panthawi imeneyi.

 18. Kaye chinkhopecho simfitinso imeneyi? amatani usiku ngati kuli kutanganidwako oyamba ndiyeyo kumalawiko ndipo zogona mu plmt mkoyamba ine kuzimva mkulu ameneyu zipangizo zina mthupi mwake sizili bwino akufunika operation pachakuti pake. Wangozijudula ameneyo ndiwokaramba. !!

 19. I see this in two ways, its either Bwana Chaponda was too much tired coz this was after the opening of trade fair in blantyre the previous day….these ppo samagona kuli president nawonso komko OR The President speech was sending the MPs into deep sleep may b due to lack of substance, or it was an empty speech. Whatever the case parliament is an honourable house and shud b given all the respect it deserves of which sleeping inside it, is not one of them.

 20. Minister kugona President akulankhula… koma bwanji inuyo anduna mutapeza junior civil servant akugona zitha bwanji? Please Check!

 21. When you grow old and you don’t want to accept it and handover responsibilities to the youth!old people need alot of rest,but you will still find very old people stil bizzy with cosmetics!

 22. Its not very strange, I have seen some presidents sleep during meetings e.g mugabe etc…. so why not him

 23. mwina anayaka, bawa ilibe ulemu, a guy of his caliber can nt sleep on a function he has spent sleepless to come out. just imagine busy signal akagone pa stage akudikira kuti amenye sound. to mi it doesnt ring any bells.

 24. In an important meeting like that one, there’s no way one is suppose to fall asleep. Kodi usiku sagona ku nyumba kwawo? Zinazi mukamalemba enanu, nkumadzifunsa kaye. Munthu aliyense ali ndi nyumba koti azikagona usiku. Nanga mpaka kugona mu Parliament, pomwe zokambirana zili mkati?

 25. Sndkupezapo Chfukwa Apapa Ngat Satana Amalowerera Ku Chpembezo Anthu Kumagona Kumaseweretsa Ma 4n Kumangotuluka Tuluka Panja Nde Mukat Kunyumba Ya Malamulo Ziwanda Zili Tho!Konko Enanso Mazko Awo Ali Kusi Kwa Nyanja Mmm Sizachlendo Izi.Mbuli Ndwe Walembawe Kuli Zofuna Kuziwitsa Anthu Kunjaku Osati Zopeperaz.Kumeneku Ndkulipepusa Zko Lanu Nde Choncho Azkukhuthuliran Maufulu Atola Nkhan Opanda Ulemu Ngat Inu.Ndwe Opepera Ndpo Uzmu Ulibe Awa Ndmakolo Ako Sukanawatero.Shame

 26. Mmmmm….kusowa zoposta eti!!!…ndani amene sawozera???…thupi limatopa..izi zitha kuchitikira aliyese!!..munangonkhumba chapondayo!!

 27. Guys tisanathawe chilungamo, a chaponda a flopper and kumagona while th przdnt z delivering hs speech and him being th leader of opposition[a newly appointed 1] shows disrespect to th whole august house and to th head of state or is t tht H.E speech was uselless. all of people why chaponda? tulo lilibe ulemu!

 28. Ngangazi sizothandiza koma zinzikatsongorera kumanda kumudzi ,zidzukulu kumudzi kwawo nzikuchula agogo anthu ena pomwe iye kumagana .amaonakhatiwafikakwawo chibwana eti kkkkkkkk!

 29. kenako muva kuti Ng’ona ya mu cup yamumeza, sangatilande u leader of the house ife anthu aku nsanje asatizolowere anyaphaphi amenewa

 30. Malo ochezera..ma s tupid people
  .ndiye ameneo..chaka chovota chikafka inu ndine ndiakaxathu mkumaty bomaaaa..disgusting ..malawi z gud bt iwe ndinngate mxika xamalawi titanipo…

 31. For me I don’t blame this man bcos he is old, I blame those who voted For this old man. Gogo (sekulu) namzukulu winu nkhumukhumbirani #turo tuwemeeeeeeee

  1. Eya and you remember bingu atangomwalira chaponda colapsed ndikuchita stroke koma ndalama brought him back to normal,those are diehards of dpp anyway kodi lucy jali alipo?

 32. Pali zifukwa zambili zomwe zingamupangise munthu kugona sizachilendo ayi komano kungowapempha aphungu athu kuti apewe kutelo kuti zazitha kusatira bwino zochitika nyumba yamalamulo

 33. Tsopano Kugona Analakwitsa? Amalawi takhalani ndi chidwi pa dzithu za chitukuko wotsati zatu mukunenazi,pali zochitika zambiri zofuna kuwunikilana ngati a Malawi Koma basi nganga amagona ,amagona wachaini? Malawi tikhala tikutsalila chifukwa mkhalidwe wongofuna kumtezela mzanthu zifukwa basi.

 34. kugona tulo n’kulinga utakhuta.akhuta ndrama zamisonkho yathu ayiwala kt tawatuma kt akoze mavuto agwa pakati pamalawi.TIKUMBUTSANE KT munthu akagona palibe chomwe amaganiza,palibe chomwe amaona,ndipo palibe chomwe amava. ena amati anthu olemera satamba nanga awa usiku amatani?.ukapanda mano osaswa phale ngati zatopetsa sizokakamiza kupuma ndibwino.nanga izi nizinthu NDUNA YOONA ZAULIMI CHOSECHO MALAWI ALI NDI NJALA WINA NKUMAGONA?

  1. sure “fort” finder I just found the “fort” in your forty spelling …. but its no big fault

 35. Kunena chilungamo ndidyera chabe anthuwa atopa,#Geoge chaponda,#Goodwell godwe,ndi ena ambiri akapume please please …..akazagwa muparliament ine sizamva chisono,i promise!!!!

 36. Nkhani ndi yoti akula akapume adzikalera zidzukulu. Ngati boma limwelo limati munthu akafika 60 yes akapume (retire) koma kundale azigogo amakakamilabe mwaona zitsatila zake .Big up reporters akamagona dziwajambulani chomcho ife tidziwauza chilungano .Mwakalamba madala kapumeni

 37. Zikutanhtauza dyera la mkhalamba zathuzi pokanilira maudindo,achinyamatafe ndi atsogoleri amawatu paja osamayiwala.Ndiye munthu akagona amathatu kuziphwitsira…ndiye sekishon 100000/1 yaMalamulo adziko lathu imati kuphwitsa pagulu ndi mulandutu….adzapeza polekera atavekedwa chibangiri..kkkkkkk koma kumenko!!!!!

 38. Zikutanhtauza dyera la mkhalamba zathuzi pokanilira maudindo,achinyamatafe ndi atsogoleri amawatu paja osamayiwala.Ndiye munthu akagona amathatu kuziphwitsira…ndiye sekishon 100000/1 yaMalamulo adziko lathu imati kuphwitsa pagulu ndi mulandutu….adzapeza polekera atavekedwa chibangiri..kkkkkkk koma kumenko!!!!!

 39. Eeeeeeee ndibwino mungosiya kulemba nkhani chimene mumadziwa kulemba ndi ma mistake basi mbuzi!!! za atolankhani

 40. Amen Mukumunen Wapanga Post Khaniy Ithink Vut Ndinuy,inu Mutamupez Mlonda Wanu Pagate Utsiku Akugon Mungamutan?Kod Atamufus Zomw Anayakhur Big Angalosore

 41. Amen Mukumunen Wapanga Post Khaniy Ithink Vut Ndinuy,inu Mutamupez Mlonda Wanu Pagate Utsiku Akugon Mungamutan?Kod Atamufus Zomw Anayakhur Big Angalosore

 42. Langa ndi mfunso ngati iwowa akugona pamene abwana awo akuyankhula ndiye akakhala ku ufesi kwawoko amagona mwamtundu wanji??? si amachita kufunda Blangeti?? nd chifukwa chake MALAWI sakutukuka anthu mma ofesimu akungokhalira kugona tifuniranjinso umboni wina apa!!!!!!!

 43. Langa ndi mfunso ngati iwowa akugona pamene abwana awo akuyankhula ndiye akakhala ku ufesi kwawoko amagona mwamtundu wanji??? si amachita kufunda Blangeti?? nd chifukwa chake MALAWI sakutukuka anthu mma ofesimu akungokhalira kugona tifuniranjinso umboni wina apa!!!!!!!

 44. Using TAX payers money dreaming? Kamuzu would have kicked this mediocre minister out of parliament & jailed for life for missusing TAX PAYERS MONEY;

 45. Using TAX payers money dreaming? Kamuzu would have kicked this mediocre minister out of parliament & jailed for life for missusing TAX PAYERS MONEY;

  1. No musamuikile kumbuyo muziganiza mchifukwa chake Malawi sakutukuka chifukwa cha anthu ngat samayenera kugola cz kumeneko ndi parliament kokambilana kayendetsedwe kadziko and anasinkhidwa kukatumikila anthu not kukagona, kod pakanatulutsidwa bill yot agulitse Lake Malawi mukuganiza kut sikanadutsa iye ali mtulo opanda kuikapo maganazo ake choncho mkumat Malawi angasinthe? Ichi mchifukwa ndinaganiza zochoka ku Malawi chifukwa ndi dziko la anthu ogona

 46. Konseku mkukakamila mpando ,anthu oyenela kupuma ntchito sakulola kuti ana omwe amaliza school aggwireko ntchito .

 47. Konseku mkukakamila mpando ,anthu oyenela kupuma ntchito sakulola kuti ana omwe amaliza school aggwireko ntchito .

 48. Kkkkkkkkk kusonyeza dziko lawufulu,amakambilanaso zawufulu, ndiye kugonakotu…..mayiko ngti,Nigeria, Egypt, Mali, Mozambique, sakanagona ameneyo. Koma mayiko onse kuli mtendele kwa Africa hvuto logona kunyumba yamalamulo mukakalipeza is normal

 49. Kkkkkkkkk kusonyeza dziko lawufulu,amakambilanaso zawufulu, ndiye kugonakotu…..mayiko ngti,Nigeria, Egypt, Mali, Mozambique, sakanagona ameneyo. Koma mayiko onse kuli mtendele kwa Africa hvuto logona kunyumba yamalamulo mukakalipeza is normal

 50. palibepo nkhani apa, tulo lilibe dolo, anyone can fall asleep anywhere anytime even while driving ngati thupi lafuna kutero, maybe sanagone mokwanira nit b4 as he is a buzy man or else samamva bwino m’nthupi

 51. palibepo nkhani apa, tulo lilibe dolo, anyone can fall asleep anywhere anytime even while driving ngati thupi lafuna kutero, maybe sanagone mokwanira nit b4 as he is a buzy man or else samamva bwino m’nthupi

 52. Guys choyamba moni kwa onse amene amakhala ndichidwi ndi Fb. Kodi simunaone munthu akugona muchurch ngakhale muzikiti nthawi imene busa or sheikh akulalikira? Tiyeni amalawi tonse tigwirane manja ndikusiya kulozana chala mwalo mogazila dziko lathu kuti mwina likhale lofanana ndimaiko ena amene anali osauka koma chifukwa cholimbikira lero ndi olemela.

  1. Kumatengera munthuyo mwina anali ndi Ntchito zina zokhuzana ndi Boma ndiye kutopa ndikutopa basi. Gays wanthuwa andalewa samagona ngati timagonera enaa ife opanda zochita.

 53. Aaaaa zopanda mchele zaziii basi kugonaso ndichani amalawi kusowa zokamba kkkkkkkkkk Chiponda 4ver Uzeugugele khona house of assembly siyakutsadza chaponda and naleparty yakho siyayifeva

 54. olembayoso mkape popeza satopako nthawi zambili mumaona ngati anthu ngati amenewa amakhala ndimpata ogona eti? Iweyo ukuti pakufunika achinyamatawe kalowetu ku parliament ngati ukuona ngati zimakhala zacisawawa, Kaya zilikomko zisatikhuze ndinkhani yogona yanuyo naweso ukagone ngati zikuyendele zakoyotu malipilo akhala akulowa ngakhale wagona kkkkkkkkkkk (niyaphapha nitokhula nini niyanya muyekeleni chaponda sikhatsi sakhe leso ayikho lento yenu) Chaponda 4ver kkkkk

 55. Chaponda alibe vuto komano vuto ndiloti kunalibeko entertainer nxt tym muxayitane Gwaladi azizayimbako few minutes then kupitilixa ma program choncho simuzawonasa wina akugona

 56. Zinaz Zimandidabwitsa Kut Kod Walemba Nkhaniwe Siudasinzeko Penapake Mot Ndizachilendo Zimenez Ndipo Anthuwa Ndi Akulu Mu Mslnkhu Osamalemba Zomwe Mr Ibu Amakamba Bwanji Busy Kutiuza Mbwelela Zanuzo, Kunali Kwa Bwino Asamakulolezen Kulowa Mnyumbai Chifukwa Zikuonetsa Kut Mwaiwala Chomwe Mumalowela Mu Nyumbai

 57. Chaponda is human there’s nothing sleep in parliament that is his house, he’s like a cat,cat sleeps anywhere,(kwa amene munawelengapo mabuku a m’mbuyomo)you can agree with me.

 58. Kodi zikutathauza kt munthu akakhala leader ov the house sagona pagulu lamulo likutelo? kapena amagona ndi iye yekha? ndimakaikila ngt tingatukuke if we ll be pointing on mistakes ife tiziva zoti Chaponda amagona?

 59. Usiku samagona kuti akagone ku pariament ngati atopa asiye ntchito anthu ambili mbili anaphunzila alibe ntchito, ntchito akuzipeza anthu akuti anatha mphamvu ngati iyeyo ndi phungu akapita ku pariament amagona akuwaudza kuti chani akudela lake si akuthandiza ayi akapumule

 60. Leader of de house falling asleep is the same as the entire house was asleep,i cn imagine how boring the speech could be. His first day as a leader could nt be like that,the boss’s speech here was really empty.

 61. Journalits trying to put jobs of cameramen under the knife as you did to presidential guard when he (muthalika) fell down after stepping on a slippery brick

 62. Ndakhala ndikunena nthawizambili kuti boma ili lidadzaza ndizianthu zamkonono lero siizimwadzionera nokha magogowa satithangata mdziko muno achoke akapume

  1. Ngati Ndichomcho.Akamapuma Onse Okalamba Chilichonse Chomwe Ndichakale Muchigwese Kaya Ndi Radio,tv Station,mitengo,cars,misinje,nyanga Kenako Uyikemo Zako Zatsopano Zoti Mulamulire Ndi Achinyamata Anuwo.

  2. Ngati Ndichomcho.Akamapuma Onse Okalamba Chilichonse Chomwe Ndichakale Muchigwese Kaya Ndi Radio,tv Station,mitengo,cars,misinje,nyanga Kenako Uyikemo Zako Zatsopano Zoti Mulamulire Ndi Achinyamata Anuwo.

  3. Stupid point opuma amatenga zinthu anapanga ,kupuma means u have done ur part now its others to continue from wer u left azagwila mpaka liti? Akapumedi

  4. your right man zikapumedi zimkhalambazi nanga chonchi zitisunga izi ? ngakhale milomo yakeyo wachita kuyilonga bwino tulo lakoma

 63. He was not sleeping but was just pretending to sleep because the address of the president was boring.He new that he could be ashamed if he could be listening with open eyes as the address contained full of nosense

 64. This guys worked day and night for the opening of parliament ….so let his sleeping not be an issue… It can happend to obama or even you….

 65. Please ife amalawi tikamayimira chithu cholakwika chifukwa munthuyo timamusapota sibwino tiyeni tivomeleze apa zinalakwika kugona ali pa ntchito yofunikira munthu wamkulu ndi kumagona ndikumati zithu zikuyenda ena akazuzula ndikumadana nawo mukuganiza bwanji?

 66. Chaponda as a minister and LoH anali ataiona kale speech ya Apm and read it over and over therefore it was lyk he is listening to somethng he oredy knew.

 67. Let us understand him he is a human being,let us forgive and forget, then we move forward.Remember!! guyz,to error is human.We cannot condemn each and every person on the small mistake that he or she makes then we can’t move forwad.Let us correct one’s mistake on the right manner.

  1. And you consider this a small mistake when the big man himself was delivering such an important speech??? But surely he will be forgiven.tiyende pamodzi ndi mtima umodzi!

  2. contrary to the issues being talked about here.who is to forgive?u are generous for no reason.mayb u give him ur forgiveness but i feel sleeping in parliament is as good as day light roberry.he pocketed our taxes through hefty allowances

  3. palibe chomwe walakwa apa ndi lamulo liti lomwe limaletsa munthu kugona HE akamayankhula?Nde munthuyo nayenso amatopa.why are you attacking chaponda only?yet njobvuyalema and crew were also sleeping.

  4. palibe chomwe walakwa apa ndi lamulo liti lomwe limaletsa munthu kugona HE akamayankhula?Nde munthuyo nayenso amatopa.why are you attacking chaponda only?yet njobvuyalema and crew were also sleeping.

 68. guys we can’t move forward tikamapanga concentrate pa zinthu zopanda mzeru, ndani sanagoneko ngakhale nkalasi,osamapeleka mfundo zoti zipitise dziko lathu patsogolo ngati mumatimokiladi a Malawi polemba nkhani bwaa.

  1. by the way,analandila allowance for this sleeping.remember,they are there to deliberate on many pressing issues,not dreaming of his wife.nsonkho wanga ukundipweteka heavy….

  2. If de subject is boring,students are forced to sleep, far from where am sitting I can smell that the president speak was boring perhaps with no salt,can someone sleep when Mugabe speaks?I doubt! !!Can someone sleep when Obama or Julious malema speaks?I doubt also!!our leaders must learn how to deliver a speak even if it is a prepared one.

  3. Leader of the house. Sleeping during the president’s key note address. Ndiye wina aziti ndi camzelu ici. Amalawi tikudzipondeleza tokha polola zinthu zoononga dziko. Kodi poti uli wa dpp ndiye ulole akuphele makolo ako?

  4. njovuyalema naye anagona bwanji simukusambwadza apa?he is human and nature caught him off guard,even in church munthu umatha kugona

  5. njovuyalema naye anagona bwanji simukusambwadza apa?he is human and nature caught him off guard,even in church munthu umatha kugona

  6. Ndewe mbuzi kwambili we voted this mother p*ssy to lead our country not sleeping dem Malawi sizanthekanso basi

 69. The leader of parliament caught sleeping on duty ndiye kusakhanaku kukutengera ubale kapena performance yamuthu this is one of the bad examples from our president

 70. ngat oyankhlayo albe mfundo nde mumaganiza kt anth aznvesera zoduka mutuzo??

Comments are closed.