Man fined for ‘disturbing’ President Mutharika’s convoy

Albinos Malawi

Ntcheu Magistrate’s Court Thursday ordered 35-year-old Precious Mnaso to pay a fine of K150, 000 or in default serve 18 months imprisonment with hard labour (IHL) for disturbing a President Mutharika’s convoy at Ntcheu boma.

Mutharika's convoy
Mutharika’s convoy (File)

The court heard that on May 14, 2015 around 3:00pm, Mnaso of Masitimale Village in Traditional Authority Kwataine was driving a Nissan Vanet car, registration number NU 851 from Ntcheu Boma towards Balaka at the time the presidential convoy was about of pass.

Police Prosecutor Sergeant, Madalitso Msikiti of Ntcheu Police Station told the court that a leading vehicle of the convoy hooted to warn him to drive off the road but Mnaso did not comply until the vehicle overtook him.

“Soon after the incidence, police officers who were on patrol rushed and arrested him at Petroda Service Station where he stopped after realizing that the law enforcers were looking for him,” Msikiti told the court.

In mitigation Mnaso appealed for leniency saying he committed the offence under the influence of alcohol.

He has now paid the fine.

Passing the sentence, Second Grade Magistrate, Philip Chibwana said ignoring to respect the state president is a serious offence which attracts a fine of about K800, 000 according to Section 112 Sub- Section 1 of Road Traffic Act.-Mana

Advertisement

290 Comments

 1. If we don’t have a knowledge on something it’s better to be quite than insulting own constitution. Social media is read by many and they lough to such comments. Where in the world would the convoy of the head of state be disturbed??? And left free? Credit to our security detail for being more professional in taking the culprit to judiciary ,irrespective of political podium issues of head of state security can not be compromised, let’s respect our leader’s, today its him and tomorrow only God knows, he/she will be required to be accorded same.this case can’t be compared with so called cash gate cases as its points to prove are different.

 2. Oh Malawians! You mean that you don’t realise the crime that this drunken master commited? Mind u, it was a presidential convoy, & as such it deserves enough security(this is supposed to be the case regardless of who is wearing the presidential costume). It hapns everwhere in the world! All i’m seeing from some of the comments is just baseless hatred that u have towards APM & not that the police were wrong in apprehending the drunken master! Malawians, wake up & start to think as modern day men & women!

 3. Kungoti a Malawi kudelela ndikomwe kumatipusisa, chomwe tingaziwe apa ndichakuti palibe lamulo lomati president akudusa ndiye galimoto zake ziime kuti che Mike Mvula akufuna aduse kaye,, president sangaime kudikila Q sizimatheka, tafufuzani maiko anzathu ngati zimenezi zingachitike?? Ngati chikhalidwe chathu chimatiuza kuti tisika njinga tikamadusana ndi akulu ndiye nanga president??? Tisamangozuzula president pachilichose chifukwa ndi mdani wathu.

 4. CHABWINO MUTHUYO ANALAKWISA KOMA ZIWAN KUTI ZIMENE MUKUPANGAZO NDIZOMPUSA CHIFUKWA PALI MILANDU YAMBIRI KOMA CHIFUKWA CHOKUTI UYO NDI MPHAWI LERO CHIGAMURO KODI MUMAPANGA ZITHU ZAKUMWAMBA KAPENA PASI PANO? APULESIDENT AMENE MWAM’MANGAYO NDIYE VOTI YANU YA 2019 MUZIGANIZIRE

 5. Mmmh malawi wa cash gate alipheeeee kumangolimbana ndi alimi basi,lamulo la pamalawi limagwira ntchito kwa osauka okhaokha ndithu

 6. I hate this judge what about the cashget people the people the frauld billions of money bt u dont judge this guy small claim lk this u judge he must pay the fine where he can get 150 000 kwachas who can eat this money stop judging 1 side plz all of us we under the Laws

 7. Mantha ngati kadzidzidzi tasiyanitsani pakati pachipani chimodzi ndi zipani zambiri ndiye zimene zikuchitika akufuna kuti tibwelelenso kuchipanichimodzi chija chowaopseza anthu kapena powaopsaza kudzera mukuwamanga kuti asamalankhule koma naife mutimanga ndithu sitisiilira olo mpang’o pomwe malawi ndiwatonse uyu sitingakhale mobanika ngati tili maiko aine ayi ndiye kuti tifufuzane muthalika wanuyo nthawi yonseyi adali kuti enafe tikungozindikira pompano kuti kuli nkhalamba inayake yotchedwa pitala ndiye akamamanga anthu oti awapeza azaleka mmanja alimkosi zimangani ngati masiku akutherani kulibwino kungosanzika mwamtendele

 8. Nsewu wo ndi wake Peter yo?? Mmene umkamangidwa nsewu umenewo iye Peter analiko?? Kumzumza mzika za MW bwanji? Mulungu asakhale chete

 9. Bwanji amalawi ?? Otsamavutika ndima satanic a DPP azaweluzidwa ndi mulungu komaso ndikuona posachedwa azaonongeka ngati Farao atizuza mokwana.

 10. Ngati munthu walakwisa ayenera kumangidwa.zisakomere mbuzi kugunda galu.kodi nanga akanagundidwa mmesa mukanapanga complain kut convoy ya presdent ikupha anthu!

 11. those who are criticizing must know this:
  1. woweluzayo sanatengele za mmutu mwake koma zili mmalamulo a dziko lino, komanso wachita quote k lamulolo lomwe n lili mu road traffic act. musanakomente mukawelenge kaye lamuloli kuti limati chani
  2.mlandu uli wonse ukauvomela umatha pompo pompo, imene siikuthayi ndi yoti woganizilidwawo adaikana
  3. lamulo limeneli anapanga si muthalika koma lunapangidwa kalekale evn nthawi ya kamuzu
  4. ngati lamulo limeneli lakuipilani muuze MP wanu akalichotse ku parliamenti
  amene amapeza mlandu woti ampatse munthu ndi apolisi otengela milandu kukhoti, akhoti amangoona ngati maumboni omwe alipo akugwilizanadi ndi mlanduwu
  5. nobody is above the law

  Chonde tileke kukomenta pa zinthu zimene sitikuzidziwa bwino

  1. Inu, what happened to the one who hit the then VP Joyce Banda at Salima turnoff? Kumanena chilungamo ndibwino. Mwina mwaiwala eti.

 12. The court heard that on May 14, 2015 around 3:00pm, Mnaso of Masitimale Village in Traditional Authority Kwataine was driving a Nissan Vanet car, registration number NU 851 from Ntcheu Boma towards Balaka at the time the presidential convoy was about of pass. Police Prosecutor Sergeant, Madalitso Msikiti of Ntcheu Police Station told the court that a leading vehicle of the convoy hooted to warn him to drive off the road but Mnaso did not comply until the vehicle overtook him. “Soon after the incidence, police officers who were on patrol rushed and arrested him at Petroda Service Station where he stopped after realizing that the law enforcers were looking for him,” Msikiti told the court. In mitigation Mnaso appealed for leniency saying he committed the offence under the influence of alcohol. He has now paid the fine. Passing the sentence, Second Grade Magistrate, Philip Chibwana said ignoring to respect the state president is a serious offence which attracts a fine of about K800, 000 according to Section 112 Sub- Section 1 of Road Traffic Act.-Mana

 13. Asilikali anali kuti osamuombera nkupheratu munthu ameneyo?amalawi mukujaila kunyoza mtsogoleri wanu.dnt try it here in Cambodia

 14. Penanso apolice mukuzitengera pamphumi inso lamulungu lapitali pawenela anandiyimitsa m’paka 2hrs kundiuzansi zimitsa galimoto lako bwampini akufuna kudutsapo. Tinangomuwona anali wapolice wa chizimayi wonenepa woyera ngati chindazi tidzawonetsana tsikundilimodzi

 15. Akalephera a save basi tsogoleri amayenera kulemekezedwa osamaphwaketsa atsogoleri,ine siwandale kma kumalawi kuno kuli umbuli kwabasi,nthawi ya kamuzu olo munthu kungotchula dzina loti kamuzu wa youth akumva uli mmadzi,ndiye mukanene tsogoleri akudutsa mkumapanga masewera anjatidwe basi ena atengere phunziro,amene akunyozawo chigamulocho nga ma 90’s zoti tathamangitsidwa ndi ma khadi sakudziwa,munthu kumangidwa cha ndege ngati waba kuli kusadula nsonkho kapena khadi ndiye muti chiyani inu (mcp era kkk)

  1. Amwene Imeneyo Inali Nthawi Ya Chipan Chimodz (One Party System) Pano Tili Mu Multiparty Komanso Ufulu Kalelo Zinakula Ndi Nkhanza Ndipo Palibe Boma Lizalamulenso Mwa Nkhanza Ngat Kale Lanulo Anthu Anali Asadapenye Pano Adapenya, Ndiponso Kamuzu Adapanga Zazikulu Mdziko Muno Zomwe Enawa Sangapange Nanga Peteryu Wapanga Chan Kut Tidzimulemekeza Manyaka Apresident Ngatameneuja Tapitan Ku City Center Mukaone Ma Bulding Akamuzu Akusowa Kupangidwa Maintainance Tidzit Sakuona Kapena Akufuna Kamuzu Akadzuke KuwakonzeraNdie Amwene Kamuzu Timamulemekeza Coz Anali Tate Okonda Malaw Osat Mbava Zalerozi Ai Ause Mu Mtendere Peter Ause Mmavuto Ndi Kumoto Osatha

  2. Indeed umbuli ndiosayamba kumalawi and like or not you are one of them, iwe ndiye mbuli yeniyeni yosaziwa komwe ikupita. Stupid man, stop defending leaders who have falled our people are straggling on the ground becouse of such leaders.

  3. Kodi naye inali mbava panthawiyo olo anapanga zazikulu kma panalibe adakamuyankhula,ndiye pano ngati mukuti anthunu ndiinu openya akumakuberani bwanji muli chipenyere kkkkkkkamene amaponyedwa kwa ng’ona aja mumadziwa kuti amalakwa chiyani,achina matenje,chiwanga ndi gadama mumadziwa chinawaphetsa,musayembekezere kuti kudzabwera mu democrancy mu tsogoleri osaba,pano akuoneka nsanga chifukwa kuli mabungwe amene akumafufuza,mbuyo muja kunalibe amati fwiiiii

  4. Dzete sakudziwika pakati paiwe ndiine,olo mutamunyoza chantundu wanji ndiye chikusintha ndichiyani ndiye udzetewo,mbutuma kupanga chinthu chopanda tsogolo

  5. Nanu a hastings chifukwa kamuzu ndi a name hahahahaha bola wati stupid man wayankhula chizungu kma iwe chindere,dzete,mbutuma yeniyeniudakakhala wanzeru udakangonena maganizo ako pankhani imeneyi osati kukhala against maganizo azako ndiye kusazindikirako kuti malawi 24 cholinga chawo akamatumiza nkhani chimakhala chiyani?anthu atumize maganizo awo,ndiye sikuti maganizo angakhale ofanana mudakali mtulobe dzukani kunja kunacha uku.

  6. Who is APM kwa inuyo? Anthu akupanga disturb Zuma, ndiye peter ndindani? Ulamulilo opusa basi, zimenezi ndi zoti munthu wanzeru angasekelele?

  7. Amartin put your coment not against someone’s coment it will be nothing bro if you are wise enough than me,don’t think everyone can think how you are thinking,this is democrancy,had been your wise enough,you can’t ask such kind of guestion,who is apm to me?it means you don’t know him,apm is the president of the republic of malawi,regardless the situation we are passing through,the solutions to these problems can only come from our maker,not any president,believe me everyone have his/her problems,checkout if any of the former head of state leave state house without any problem,xool me.

 16. petera ndi mphawi zoona kukongola ndalama ku munthu wakumuz,,,,,,,,,,,,,, ena mkumapanga ma coments otiopseza kut atimanga ctikuopa tikufuna kupanga malawi wabwino,,,, olo atimange atimangira pa choonad ,,,,,,, ndezichepe zomaopsezana coz kut afike pomwe alipo ndife amphaw amene tinachita kumunyamulilapo

 17. Kunaliazao Kumuzu , Ana onse aschool timapita ku sanjika kumakayimba manja , komaiye ali kuzomba sayamuke .and true disturbing our business

 18. He make a good history , reason the law doesn`t allowed such move on front the president. Please try to respect the leader of today &tomorrow

 19. Ife monga angoni apaphata tisamutsa judge ameneyo asawonenso madala wanthu .komanso nseu umenewu adaukonza ndi kamuzu pasapezeke ochuluka nzeru .

 20. All of them should be fined for disturbing each other. Mutharika must pay k3 000 000 000 00 to a man because he is rich, and a man must pay k150 000 00 as mentioned on the statement

 21. Mmmmm nawo amachita kuonjeza kuyenda munseu wa busy alibe helicopter kodi koma galimoto za police ziimitsa anthu nawo samaganiziza amapeka magalimoto awo a president sananyamuke ku nyumba ya boma yawoyo ndiye kuti apolicewa ayenda kale ulendo wa 3hrz kuimitsa anthu kumbali ena nawonso akuyendera zofunikira pompo pamenepa a president ndi amene amasokoneza anthu pamseu kudikira kowawa matha ake a mtundu wanji sangamayenda mbali imodzi anzao nawonso azipeza mpata udutsa nao malinga ndi umphawi wamiseu ulipo kwathuko komanso choti adziwe #Mr_President’wo a busy si okha aliyense ngati ali pamseu ndiye kuti ali busy kuphelerana ufulu kumeneko wamayendedwa pamseu

 22. zina ukamva kambanga mwala.iwe mutharika sumadziwa kuti Nawenso umapanga Disturb anthu komakuti amangokupilila?osapanga vutto losapanga misewu yokwanilatu ndi limenelo kapena nanga osamangoyennda pandege bwanji ngati mmene amkapangila okuba mzako wina uja?ngati zinagulitsidwa Gula ina ndege yoti uziyendera zachamba basi.ndichifukwa chani osawukafe mulanduwathu suchedwa ku weruzidwa?nawe iwe waweluzawe wagwiritsa ntchito lamulo liti kuti mwinanso yemwe atazaweruze ya cash gate atenge lomwero la pompopompolo.oweruzawe dikila poti nawe wasala pang`ono kuti mulungu azakuwerula ndi mutharika wakoyo.

 23. This is stupid …aziyenda pakabaza ..anzao anasiya kuyenda pagalimoto nzele kuno ndi uko pompa pa tanzania pa president ama kwera njika ….ndemukamange munthu pazifukwa zake zimenezi ……

 24. Enanu umbuli ukuphani mulibe manyazi zotukwana zimatinyasa muzitukwana makolo anu ife peter timamukonda mukhalira zomwezo zotukwana

 25. Kulemekeza mdipiti wa galimoto za Mtsogoleri wadziko sizinayambe lero…Ndiye ngati wina kukhuta mowa(mmene wanenera mwiniwakeyo) ndikusapatuka?ikanakhala ambulance bola.Ndalamayo ikukwanira mwinanso nkuganiza zosiya bibida.Koma ndi mwana osanja eti…pompo phaphapha ….mulu ndu!!!kulipira?anthu mukulimba eti

 26. Kulemekeza mdipiti wa galimoto za Mtsogoleri wadziko sizinayambe lero…Ndiye ngati wina kukhuta mowa(mmene wanenera mwiniwakeyo) ndikusapatuka?ikanakhala ambulance bola.Ndalamayo ikukwanira mwinanso nkuganiza zosiya bibida.Koma ndi mwana osanja eti…pompo phaphapha ….mulu ndu!!!kulipira?anthu mukulimba eti

 27. Kkk ma judge aku Malawi, mulandu wa Muluzi ukukanika amanga munthu kamba kodusa museu, agalu kwambili, Muthalika ngosaukadi anabwela kuzalemela ku Malawi kkkkk, kumanka kumatolela Ma 150, galu wamunthu

 28. No one above de law koma apa zaonjeza 3days mwambo wamulandu watha kale coz ndi poor man pomwee aja anaba ndalama pano zikutha zakazaka osagamula koma muli ndi umunthu? apadi ndakhulupilila kuti kukhala malawi ndikulimba mtimba ndipo kobadwila sitinasange! mwayamba kutenga malamulo amugabe kubwelesa kwathuko mmmmm (Tikamalila by Lucius banda)

 29. He deserve it cos ena amanyanya matama. Ulemu ngofunika kwa President ayaa. Inefe tinakhala 4hours tilipamzere kuti timuvotere amayoo timamkonda

 30. Ithink ambiri amene akunyoza chigamulochi abadwa zaka za mma 2000, Tikukumvetsani. U dont know wht u are saying. Chifukwa nthawi ya kamuzu makolo anu amasanjana munsewu kamuzu wa mcp akamadutsa.

  1. Man mukunena bwino inu nthawi yendani ya kamuzu ino ndi nthawi yazipani zambiri asatipangeso ngati tilimuchipani chimodzi ai ndi nthawi ino yomasuka yosafuna kukhala omangikaso wamva bwanawe

  2. Kulibe kupanga zasopano,, sizololedwa kumasewela munsewu pamene president akudusa, palibe dziko limene lingamalolele zopusazo zikuchitika

  3. kkkkk.. So demokalase means no more presidential prevelages… or respect… muziganiza muli inu.. mungonena….. anyway….ngakhale kuli demokalase mmalamulo adzikp lino zimenezo zirimo. Ndipo anachita dala chifukwa. anadziwa kuti pazapezeka anthu ngati inu ofuna kumupepusa mtsogoleri wadziko kuti akhale ngati oyimba, beru pachalichi cha ku ntchenantchena…. So multiparty is not equal to indiscipline… otherwise the remainder will be prison/fines as the case with the case in ntcheu…

  4. Yassin Tsekula Maso Ako Nupenye Kamuzu Si Mbava Ngat Peter Ndi Anthu Awili Osiyana Kamuzu Adatukula Dziko Lino Vuto Ndi Akumipando Nkhanza So Inalinso Nthaw Ya 1party Pano Kuli Ufulu Zomwe Apanga Aboma Pogamula 150 Ndizopangisa Kut Amalawife Basi Tizingosauka , Osamabeleka Mbuzi Kumbuyo Ai Ngakhale Ali President Iyi Ndi Njira Imodz Yowonetsa Kukwiya Kwathu Peter Mbuzi Ya Munthu Ya Kuzimbabwe

  5. Miseu yakenso imene akuti amanga disturb yo ngati miseu yeniyeni, anzanu amamanga miseu ikuluikulu palibe zoimitsana president akamadutsa , timangompatsa lane yake kt adutse sizopusa zimene mukunenazi

 31. Kungounikirana mtsogoleri amayenera kukhala: 1-Wachisoni 2-Okhululuka 3-Waulemu 4-Omvetsetsa 5-Odekha 6-Okonda anthu wake Ndi zina zotero………………. Nanga kodi #PITALA cholinga chako nchiani kufuko la #Nyasaland?

 32. Ameneyo ndiye fodya wosutira kuchimbudzi, Zankhutu, popanga zimenezo mdxiyamba mwanganiza kaye, mkutheka munthuyonso adakuwinitsa kuti mufike pamene mulipo ndi vote yake, lero vote yake inja yamutembenukira. Mwina mukupangira Chikuwawe powona kuti ndiwachingawo chapakati ndiye mkutheka kuti wa chipani Cha MCP? Mudzafa Imfa Yowawa ndinthu.

 33. Apa mulandu ukanakha oyendetsa galimoto atamwa mowa basi osati zinazo. Pokha pokha akanapangitsa ngozi pakanamveka.

 34. ndithokoze ma judge a ku malawi pa changu chomwe ali nacho pa milandu yaing’ono/yopanda ntchito kusiya ikulu ikulu ikungogonekera popeza amakhala atadyesedwa chintuwisa. ndakwiya nanu.

 35. eeee apa nde ndaziwa wabwino ndimulungu ekha kod guyz mulungu tansokoneza kangat mujila zake zabwino ife mkumafuna zoipa kod atati atigamule tingapeleke ndalama zingat nanga atat atimange angatimange zaka zingat

 36. Ngati ulibe chonena ndibwino kukhala osatulutsa mau, awa aboma kuti ayambe kukutsaka ndi m’mamawa womwe akupeza. Ndiye ukafuna kuti ukhale wanzeru tiye pitilliza, koma akakupeza mawa usadandaule ndi bomatu iyi.

  1. Boma ndani, muuzane mukasake anapha Chasowa ndi Njauju.Akuba ndalama zaboma mukuwabisa. Ukasake anaba maTractors.Kufuna kupha ndi kumanga zimene uziwa iwe .Tikufuna Chitukuku ife,zomangana ndi zakuphana ife ayi.

  2. Ndiye chimene ukutsutsa ndi chiyani pamenepa, popeza wekha ukudziwa kuti anamupha chasowa ndiye chingavute ndi chiyani kukupeza fisi ngati iwe? Ukuona ngati, zingawatengere nthawi atayamba kukusaka.

  3. Chitatu makani ako, uwone Jombo ikubwera kunyetsa matako akowo uhule wako alankhulawo ukuthere ukuona. Ndiwenso ndani, mdima ukakula dziwa kuti kwatsala pang’ono kucha pitiliza uwone zosaona. Tione ngati, malume ako angakatsumire amene akuwanyozawo.

  4. Why shud pple fail to give xere views bcoz of fear? We cant..xis z a democratic nation..we r no longer leaving in dark ages Mr. Am very sory for u u boot licker…

  5. Mfana ndwe #bombocrat,,,boma lizisaka mu2 chifukwa cha comment pa fb mmalo mosaka a2 opha ma alubino,,,i thnk cholemba changokusowa or mwna watumidwa

  6. iweo kudya zabomazo chani?u thnk we can b scared with dis stupid goverment?osamathana ndi njalayi bwa but bzy ndi munthu oti palibe chomwe angapeze mwa iye, iwe jaafaalii i thnk ua stupid as ua govermrnt

  7. Had it bn that many ppo includng Chilembwe, Kamuzu and Bakili had the feeling like yours Jafali tnakakhala kuti ndife akopolobe mpaka pano. Fear Not coz sbwno kumata pakamwa ukuzwa truethness ya nkhan, Change your mind as the world is changing.

  8. Nonsense and your stupid fool tell them to look after people with Albinism, Maize and all those poor orphans who wandering in town,thats why you and your stupid government failed us.Osaopa part 3,kauzaneni foolish

  9. Kod John Chilembwe Akadaopa Kufa Tikadapeza Mtendere? #Jafali Ndimaona Ngat Ndiwe Msilamu2 Koma Coz Msilamu Amalimba Mtima Ndipo Amwene Mukapanda Kuima Pa Chilungamo Powopa Wina Muzafa Ndipo Osakawo Ayambepo Peter Ndi Iwe Khwangwalawe Machende Anu !

 37. inever see any car stop president mzuma akamadutsa koma kumalawi convoy ili pa zalewa koma ku lunzu magalimoto aimitsidwa kale koma boma la pitala lokha

 38. Check in, in Mzansi please president convoy ndi anthu wamba amayendera limodzi pa nsewu ndi Maliro okha omwe anthu amapereka ulemu ndiye ulemu wanu a president mungopanga extend m’misewu basi ndipo fine mwapereka kwa mphawi mzathuyo simudzaperekanso ayi mwalo mwake mudzalandira ulemu

  1. Jeyne Wosadandaula iwe khala pa low ndikupulumutsa kwa woipayo poti satana naye watsikira ku Ndata kuti ense wolambira muthalika akathe kumakhala ndimatha m’dziko lake lomwe.

 39. Ngati anthu akumagwada ena kuthawa kumene akaona ma galimoto ama satanic profet mtownimu nde wina akasokoneze the whole president??? Amangidwe basi

 40. shame!..President being protected than Malawi itself…fools…infact pigs…swine is d other name…poor ppo aren’t your cusions…fined-fined or 18 months IHL my foot!

 41. stupid judge and government, mulandu wadzulo lero chigamulo oba ndalama zaboma angokhala no judgement mpaka chaka chachitatu

  1. Ndipo Mnyero Wako Mwina Ndiwe Mchewa Kumtumbo Kwako Wekha Siukuona Kut Akubela Osauka Pamenepo Mbolo Yako Ndi Machende Omwe Mxiiiiiuuuww!

  1. Iye Akudana Ndi Munthu Kusiya Momwe Watisokonezela Dzikomu Koma Mr Ibu 2019 Udzivotela Wekha Iwe Tione Ngat Uwine Galu Iwe Nanenso Zandimange Sindakutukwana Foreighner Iwe

 42. aaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaaah sibwino chancho aaaaaaaaa moyodi ndiokondera bwanj

Comments are closed.