Breaking: Muluzi’s co-accused, Lyness Whiskey, collapses in Court

Advertisement
Bakili Muluzi

Second accused in former Malawi President Bakili Muluzi’s  K1.7 bllion corruption case Lyness Whiskey has collapsed in Blantyre high court today.

Bakili Muluzi
Bakili Muluzi’s co accused collapses

According to Judiciary Spokesperson Mlenga Mvula Whiskey started gasping as soon as she got locked in the dock for cross examination this morning.

“I can confirm that she collapsed this morning and she was taken to Blantyre Adventist Hospital for medication” said Mvula.

Whyskey was Bakili Muluzi’s personal assistant. The former Malawi leader is accused of misappropriating over K1.7 billion when he was in power.

The case has stayed on judicial desks for over ten years due Muluzi ailing situation that deteriorates the moment he is taken to court.

Blantyre High Court judge, MacLean Kamwambe, has vowed to bring the trial to its finishing point. But following Lyness Whiskey’s collapse, the judge adjourned the case to Tuesday 19 April 2016.

Advertisement

198 Comments

 1. zanu izo kumeneko ndikumtunda abwana bakili samanama palibe kuzengana mulandu apa zachamba mumu siye anadyazake kale ameneyo zitsilu zadpp usova peter tchende lako kumene uliko

 2. This movie is taking so long to come to an end, this scene has gone that way and you are now telling us to wait for the next episode, roll! keep on fooling us but from a distance God is watching. If lucky is with you then we are not lucky. You are drinking expensive bottled water as you are waiting for the proceeding yet masses out there are queueing for a pale of water at a kiosk with dry taps. God save mother Malawi.

 3. Kkkkkkkkkkkk! Wagwa nayo wina mu court! Ndili Ine judge ndikadangogamula kuti anthuwa ndiwolakwa basi apite ku ndende. That’s a sign of guilty! Munthu wosachimwa sanjenjemela, amayankha mtima uli ziiiii! Tsano mpakana kugwaaaaaa? Wht more evidence can the judge need here? Must she die then?

 4. Kkkkkkkkkkkk! Wagwa nayo wina mu court! Ndili Ine judge ndikadangogamula kuti anthuwa ndiwolakwa basi apite ku ndende. That’s a sign of guilty! Munthu wosachimwa sanjenjemela, amayankha mtima uli ziiiii! Tsano mpakana kugwaaaaaa? Wht more evidence can the judge need here? Must she die then?

 5. Koma ngati anthu ena mukuona ngati khanizi ndi zosewera muwafunse eni akewo mulandu suwola ndipo suchepa mkulu wina ankamuuza kuti ndalama wagula jet zoti ndizathu ndizimene amati athandizire program yodyetsa ana phala mmasukulu iye akanka mkuyamba kunyoza eni ndalama wo mkuthamangitsa kazembe wawo koma anapita pati ukalakwa Koma kupepesa mzuma anapepesa ndiye enawa ndindani timagulu tinati tizipani tinati mwationa kale tatha ndipo tikutha chifukwa chakuba zakuba ndizosadalitsidwa mpaka musauka nazo olo mwinanso kuononga thanzi lanu pepesani bwezani sikupusa onani patsogolo olo zakeyu anabweza

 6. Koma ngati anthu ena mukuona ngati khanizi ndi zosewera muwafunse eni akewo mulandu suwola ndipo suchepa mkulu wina ankamuuza kuti ndalama wagula jet zoti ndizathu ndizimene amati athandizire program yodyetsa ana phala mmasukulu iye akanka mkuyamba kunyoza eni ndalama wo mkuthamangitsa kazembe wawo koma anapita pati ukalakwa Koma kupepesa mzuma anapepesa ndiye enawa ndindani timagulu tinati tizipani tinati mwationa kale tatha ndipo tikutha chifukwa chakuba zakuba ndizosadalitsidwa mpaka musauka nazo olo mwinanso kuononga thanzi lanu pepesani bwezani sikupusa onani patsogolo olo zakeyu anabweza

 7. Inenu mukawona muthu olemela mumamutengangat mulungu ena mukumalemba ma messag bushli ndipepheleleni ndipeze chito chikhalileni sintumikiayi akanakhala opephera mucho akanaipephelera malawi ikhale yotabwi kulemelakwaji kogolemera muthumoziyekha amaliwi kupusa

 8. Inenu mukawona muthu olemela mumamutengangat mulungu ena mukumalemba ma messag bushli ndipepheleleni ndipeze chito chikhalileni sintumikiayi akanakhala opephera mucho akanaipephelera malawi ikhale yotabwi kulemelakwaji kogolemera muthumoziyekha amaliwi kupusa

 9. Voto la amalwi mumamusatila muthu wa satanic kusiya wabwino kud bushili anakupagilanichani bakili ndimuthu wapanga zazikulu pamalawi achakwamba amafuna kuphulisa malawi ndi mabomba koma bakili anatiteteza paka anamugwila zambili taziziwa ndibakli ngati ma 4ni sukulu zawulele ftelza ochipa chimangacha kenya mukuyamikila wasatanic

 10. Guys tizimvetsa don’t mix things we pple we mixing b.muluzi&cashigate atsiyeni a court agwire ntchito amene amaziwa malamulo don’t blame peter’s regime tilakwitsa let the judiciary react not president we….! Malawi come on guys iiii!??

 11. Guys tizimvetsa don’t mix things we pple we mixing b.muluzi&cashigate atsiyeni a court agwire ntchito amene amaziwa malamulo don’t blame peter’s regime tilakwitsa let the judiciary react not president we….! Malawi come on guys iiii!??

 12. Kodi Iwe Michael wuthupa ukusakaniza nkhani ya Atcheya ndi Bushiri bwanji? Kodi inenanu mumaganiza ngati nkhuku yeti ukungoti kuzikundikira chuma unamva kuti chinali cha boma? ndalama zopatsidwa ndi Gaddaf zo malemu uja anazit engera pa mgong’o. K92bn yija ingafanane ndi K1.7bn. Fotsek mbuzi michael

 13. Kodi Iwe Michael wuthupa ukusakaniza nkhani ya Atcheya ndi Bushiri bwanji? Kodi inenanu mumaganiza ngati nkhuku yeti ukungoti kuzikundikira chuma unamva kuti chinali cha boma? ndalama zopatsidwa ndi Gaddaf zo malemu uja anazit engera pa mgong’o. K92bn yija ingafanane ndi K1.7bn. Fotsek mbuzi michael

 14. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 15. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

 16. Please osamuleka…..mpaka atabweza muthu kukhala oleme pa number 3 mu africa while his people dieing due to lack of medication….no food and etc….coz 1 person shame on to those who supporting clocks mxaa!

 17. DR CRIS solve problems like Lost Lovers, Marriage Protections, Failed to find a lover, Divorce, Lost property or you want to quickly sale your property, Court cases, Business protection and success, Job Promotion, Want to get wisdom, I give supper natural powers, I stop or remove witch craft from homes businesses, I cast spells but i also i stop them, Do you want to get rich i remove curses from people and give them lack, I quicken delayed payments/ Pension.CALL /TEXT 0971622860 +260967158374 : +260967158374 / +260971622860 PAY AFTER WORK . SAME DAY RESULTS. WE DELIVER

 18. DR CRIS solve problems like Lost Lovers, Marriage Protections, Failed to find a lover, Divorce, Lost property or you want to quickly sale your property, Court cases, Business protection and success, Job Promotion, Want to get wisdom, I give supper natural powers, I stop or remove witch craft from homes businesses, I cast spells but i also i stop them, Do you want to get rich i remove curses from people and give them lack, I quicken delayed payments/ Pension.CALL /TEXT 0971622860 +260967158374 : +260967158374 / +260971622860 PAY AFTER WORK . SAME DAY RESULTS. WE DELIVER

 19. Koma odandaulawo samaziwa kuti milandu ya 1964 yomwe amawapasa amuluziyo ndiyamunthu amene anamwalira kale ?nthawi imeneyo ameneyo amalamula ndi kamuzu banda tikukumbuseni oimira boma zikomo.

 20. Koma odandaulawo samaziwa kuti milandu ya 1964 yomwe amawapasa amuluziyo ndiyamunthu amene anamwalira kale ?nthawi imeneyo ameneyo amalamula ndi kamuzu banda tikukumbuseni oimira boma zikomo.

 21. I think joice banda could have been the following foot prints of achair not peter.u r blindfoding us wit achair issue instead of dilling wit these cashgate issue.even if achair can pay back the money or being sentenced the probrem in finance wil remain increasing

 22. I think joice banda could have been the following foot prints of achair not peter.u r blindfoding us wit achair issue instead of dilling wit these cashgate issue.even if achair can pay back the money or being sentenced the probrem in finance wil remain increasing

 23. Man mukamba za Bushiri ndi nkhani alemba apayi parall Ulemelero wapasi pano ndipo kulemela kwake kusatikhudze enafe kaya ali ndi Ndege ,Malo awulele.kaya ma milion ndizake zimenezo limbikani Job mulungu azakupasani . Ife tufuna awa akupangitsa kuti Mw azisawuka kamba kozikundikila chuma chadziko makosana amenewa atati asamabe ndalama za dziko malawi sangakhale Osauka ayita .BUSHIRI NDIZAKE ZIMENEZO NAYESO ALI NDINJILA ZAKE ZOPEZELA MONEY

 24. Man mukamba za Bushiri ndi nkhani alemba apayi parall Ulemelero wapasi pano ndipo kulemela kwake kusatikhudze enafe kaya ali ndi Ndege ,Malo awulele.kaya ma milion ndizake zimenezo limbikani Job mulungu azakupasani . Ife tufuna awa akupangitsa kuti Mw azisawuka kamba kozikundikila chuma chadziko makosana amenewa atati asamabe ndalama za dziko malawi sangakhale Osauka ayita .BUSHIRI NDIZAKE ZIMENEZO NAYESO ALI NDINJILA ZAKE ZOPEZELA MONEY

 25. Un empty tin makes more noise. Chonde! A Malawi anzanga tatiyeni tizilemekezana ndi kukhala anthu akhalidwe labwino. Kuyankhula zotukwana, kunyoza wina sibwino zimaonetseratu kuti munthu ndi opanda khalidwe. Nkhani za khoti zimaweruzidwa m,mkhoti basi osati ndi anthu kunja kwa khoti. Kuti wina ali kudata chifukwa amalimbana ndi Muluzi sibwino chifukwa okondedwa ake akamamva zotelezi zimawawa

 26. Un empty tin makes more noise. Chonde! A Malawi anzanga tatiyeni tizilemekezana ndi kukhala anthu akhalidwe labwino. Kuyankhula zotukwana, kunyoza wina sibwino zimaonetseratu kuti munthu ndi opanda khalidwe. Nkhani za khoti zimaweruzidwa m,mkhoti basi osati ndi anthu kunja kwa khoti. Kuti wina ali kudata chifukwa amalimbana ndi Muluzi sibwino chifukwa okondedwa ake akamamva zotelezi zimawawa

 27. Muluzi ndimuluzi palibe angamuthe sikut wakomoka ai koma akukafusa nzeru kwa nzimu wabambo ake mr kapoloma komaso mukuziwa kale atcheya sachepera mukamufuse atupere akakuuzan

 28. Muluzi ndimuluzi palibe angamuthe sikut wakomoka ai koma akukafusa nzeru kwa nzimu wabambo ake mr kapoloma komaso mukuziwa kale atcheya sachepera mukamufuse atupere akakuuzan

 29. zomwezi mpaka ache Bushiri?? Enanuso Mudima Munakujani Eti?? Kugundika Kuzenga Aanzanu Zakuba,tizawona Nanu Mukazatula Pansi Udindowo,dziko La Malawi Mpaka Yesu Adzabwela Sirizatukukaso.

 30. Ngakhale akanakhala kuti anasokoneza K20,000.00 akuyenerabe kuyankha mlandu…mlandu suchepa.
  Komanso tisiye kulowesa ndale mu court.Panopa tikukamba za 1.7 billion panopa, ndiyomwe ili m’court..ngati zili nkhani za kubedwanso kwa ndalama zina ndi anthu ena zimenezo tidzakamba nthawi ina. Sozomakomoka dala apa ai.Pa 19 sikutali, tidikira ndithu!

 31. Kkkkkkkkkk MALAWI. You call yourselves the warm heart of Africa. Why cant you just change and instead you simply call yourselves the cold heart of Africa. Because I dont think you will become warm again. So sad!!

 32. Mbuli muuzimu. Tcheya samatekeseka ndi zazii ngati izi mukucheza, mufufuze bwino oonse amalimbana naye ena ali gooneee Ku ndata nde mukutaya nthawi Tcheya anapanga chitukuko si zamisala zanuzo mbuzi zaanthu manja ogwirana basi!!!! Salute

 33. Anthu opepela inu muzachangamuka lit zakale kale mwaiwala ma bilion anabedwa nthawi ya Bingu nankha nthawi ya Joyce bwaaaa

 34. Anthu opepela inu muzachangamuka lit zakale kale mwaiwala ma bilion anabedwa nthawi ya Bingu nankha nthawi ya Joyce bwaaaa

 35. Bushiri kuti achitepo chani? Suja inu nomwenu a Malawi mukumakana kuti simungamalandire ndalama za magazi? 2, munthu akati athandize pa mavuto omwe agwa mu dziko lathu, mukumanena kuti akufuna kuchita kampeni yoti azakhale u president? Ngati South Africa ikumupasa malu aulere kuti amangepo chi church chake, ndi masewera ngati? Munthu woti ali ndi ndege ziatu, ndi prophet wachiwiri wolemera pa Africa, ali ndi chitsime cha mafuta, ndi masewera?

 36. Bushiri kuti achitepo chani? Suja inu nomwenu a Malawi mukumakana kuti simungamalandire ndalama za magazi? 2, munthu akati athandize pa mavuto omwe agwa mu dziko lathu, mukumanena kuti akufuna kuchita kampeni yoti azakhale u president? Ngati South Africa ikumupasa malu aulere kuti amangepo chi church chake, ndi masewera ngati? Munthu woti ali ndi ndege ziatu, ndi prophet wachiwiri wolemera pa Africa, ali ndi chitsime cha mafuta, ndi masewera?

  1. Choka iwe South Africa yake iti yomwe yampatsa bushiri Malo a ulere?koma ukuwadziwa ma Zulu iwe,ukumudziwa Jacob Zuma iwe,Malo aja adagula man,Bushiri ndi mfana wa cash sikuti ndi wachiwiri mu africa usatinamize funsa T.B Joshua ndege yake yoyamba adagula mu 1994,Bushiri Ali ndi zaka 15 koma panopa T.B Joshua Ali PA number 5 mu Africa Ali ndi ndege 6,uzinamiza zitsiru kumudzi kwanu konko

 37. tikufuna 95 billions komwe anaba z DPP aja osati ka 1.7 billion ayi musaone ngati tidaiwala zonse tikukukbukila siife ana kapena openga ayi mxiiiiiii!

 38. tikufuna 95 billions komwe anaba z DPP aja osati ka 1.7 billion ayi musaone ngati tidaiwala zonse tikukukbukila siife ana kapena openga ayi mxiiiiiii!

 39. Mwanya gys ndikakumbukila kamulepo adanena kumangochi, talimbana ndigwazi ife ine atcheya agwandachakwamba achakufwa chihana aaaka kagwazi kanalipoooo

 40. Mwanya gys ndikakumbukila kamulepo adanena kumangochi, talimbana ndigwazi ife ine atcheya agwandachakwamba achakufwa chihana aaaka kagwazi kanalipoooo

 41. Kkkkkkkkk, kukalimbana ndi 1.7 billion, kusiya ma billion omwe anabedwa ochedwa Cashgate, ndiye kuti pali nzeru pamenepo? Ma billion ndi billion, chachikulu nchiti? Ndipo mulandu woyenera kuti ulowe mu khoti nsanga ndi uti? Penapake a Malawi mukumvetsa chisoni. Kaya ndi ndale za malitsiro zomwezo, kaya ndi umbuli, kaya nkutembeleredwa, sindidziwa.

 42. Kkkkkkkkk, kukalimbana ndi 1.7 billion, kusiya ma billion omwe anabedwa ochedwa Cashgate, ndiye kuti pali nzeru pamenepo? Ma billion ndi billion, chachikulu nchiti? Ndipo mulandu woyenera kuti ulowe mu khoti nsanga ndi uti? Penapake a Malawi mukumvetsa chisoni. Kaya ndi ndale za malitsiro zomwezo, kaya ndi umbuli, kaya nkutembeleredwa, sindidziwa.

  1. Man mulandu wa Bakili ndiwakale nthawi imene ankalamulira choncho watenga chinthawi usanathe. Ukukamba za Cashgate yazana zanali. Ndiye ukati boma liimbe mlandu mabillion a Cashgate kusonyeza kuti wa Bakiliwu simulandu? First thing first.

  2. Madzi Amachoka Ku Mtunda Kupita Kumusi. Pafunika Kuyamba wa:
   1 Muluzi 1.7billion
   2 Bingu Wa Muthalika 577billion+trcts
   3 Joyce Banda 13billion+ndege

   Onse amene anaba ndalamadzi alandile chilango basi akakhala peter uyu azake ammanga akazagwa chifukwa akuwoneka kuti watedza. nayewa yambaira kuba bola anzakewa amaba akupanga chutukuko, komano kanganyayi palibechiwonaine. Kaya anzanganu popedza kona kusiyana

 43. Olakwa ndi anene wakomokayo,mwina anamwa whiskey wanbiri.Kukomaka kukuotseratu kuti nkhaniyi akuidziwa.Akhoti munthuyu akazizimuka muzamufunse kuti kodi umakimokeranji?Osalakwa sakomoka amangoyankha kuti palibe chomwe ndikudziwa.

 44. Olakwa ndi anene wakomokayo,mwina anamwa whiskey wanbiri.Kukomaka kukuotseratu kuti nkhaniyi akuidziwa.Akhoti munthuyu akazizimuka muzamufunse kuti kodi umakimokeranji?Osalakwa sakomoka amangoyankha kuti palibe chomwe ndikudziwa.

 45. Ikatha ya bakili muluzi tiyambe so za cash get mbava za cash get zilowe nazoso kuka nyumba komata matako hahaha koma a malawi amati pangitsa zina awa tikungotha inki yamu phone ndiku ikapo ndemanga zo pusa apa zose ndizi ma tsotsi izi kuya mbila joyce banda?pitar wa muthalika?ndimbala bakili muluzi?ndimbala nde anyani aku sekana zikundu awa hahahahahahaha

 46. Ikatha ya bakili muluzi tiyambe so za cash get mbava za cash get zilowe nazoso kuka nyumba komata matako hahaha koma a malawi amati pangitsa zina awa tikungotha inki yamu phone ndiku ikapo ndemanga zo pusa apa zose ndizi ma tsotsi izi kuya mbila joyce banda?pitar wa muthalika?ndimbala bakili muluzi?ndimbala nde anyani aku sekana zikundu awa hahahahahahaha

 47. ABALE INU PLEASE LEAVE BAKILI ALONE, HE IS NOT THE ONLY ONE AMENE WADYA NDARAMA ZA BOMA, SOME ARE STILL ENJOYING LIFE WITHOUT BEING VICTIMIZED, WHY BAKILI? TISIYIRENI BAKILI WATHUYO TIMAMUKONDA INI AKEFE.

 48. Anthu inu ndi otani? Dikirani oweruza ampeze osalakwa ndiye azamasulidwe osati mukukambazi ayi.Andalewa akubabe chifukwa makhothi amakonderabe andalama ngati amenewa,azatayidwa.

 49. osamuleka akachira muyambirenso mulandu,ngati akufuna kuthawa mulandu afe,apobi amangidwe basi, dziko laMALAWI limadalirabe madonors chifukwa cha mbavazi.

 50. Let go people,his old now dont u have mercy.u acryn for a billion yet more billions u know the people who took it. sad midocre people

  1. Enafe tikamanena za nkhani ya cash gate amati palibe chomwe ukudziwa,nanga lelo wina wagwa bwanji mkhoti kamba ka milandu yomwe idaola kale kale?.Wina adakuthawani uyo ndipo akudya zonona komwe aliriko,koma mukulephela kumumanga ndiponso nchifukwa chake adasiya kutithandiza azunguwa chifukwa chofuna kukolola pomwe simudakhetse thukuta.Mulandu umenewo siudzatha mpaka muluzi atafa chifukwa munthuyo wakula komanso akudwala,mudzaona chomwe chidameta nkhanga mpala.

  2. The thing ndizakuti dolla imene anaba amuluzi a court sanadye nayo olo one tambala pomwe cash gate anadyesela dyesela nkona inangoti ziii apapa akufuna kumubela kandalama kenakake amuluziwa sangango musiya

  3. Manyi akale sanunkha koma apa anunkha wa cashgate ndi uwu wa 1.7billion yonse ndi milandu koma choseketsa nchakuti nkhani ikayamba timva mboni yadwala apa wina wagwera mkhoti eish ndale

  4. Matter of fact ure a out of the point, bring forward ur point of view not critising me on my english,ngati iweyo ndi nzungu or some.despite english the topic on the table is bout bakili stop westing my time moron

  5. Kkkkk ana midyomba english ine kudabwa kkkkk.inu zanu ndikusoka,uhule&kugulitsa zovala basi kkkk.swaga imafuna xool wava cassim anafi kkk.www.tipite ku jubek.com.samala kuti zeno kkkkkkk

  6. Kkkkk ana midyomba english ine kudabwa kkkkk.inu zanu ndikusoka,uhule&kugulitsa zovala basi kkkk.swaga imafuna xool wava cassim anafi kkk.www.tipite ku jubek.com.samala kuti zeno kkkkkkk

  7. Kkkkkk bola wava anafi.l think u will never write your broken engilish again.jst write chichewa pls ungathawitse mahope ako.

  8. I will never stop writtin english have u ever been in europ before.olo south muzafela konkunotu inu i have travelled before, over seas. u a not my level

  9. Yes am not yo level coz u speak broken engilish.u r de 1 mumatiipitsira mbiri kwa eni coz of yo broken engilish.pls improve.

  10. Mzimba is my work place amwene kkk kamba ina l hv been in Bt for so long.ndapanga trainnig yanga komko wava kkkkk kamba ina.

  11. Mzimba is my work place amwene kkk kamba ina l hv been in Bt for so long.ndapanga trainnig yanga komko wava kkkkk kamba ina.

Comments are closed.