Bakili wrongfully arrested

Advertisement
Muluzi

Lawyers for former president Bakili Muluzi have claimed that the former president was wrongfully arrested since the Anti-Corruption Bureau (ACB) has no evidence that the accused stole public funds.

Muluzi together with his former assistant Lyness Whiskey are accused of stealing public funds amounting to K1.7 billion.

During cross examination of the first state witness Victor Banda, Muluzi’s defence lawyer Tamanda Chokhotho argued that “It was wrong” for the ACB to arrest his client on claims that he failed to explain the source of the money which had been deposited in his personal accounts.

According to Chokotho, his client had a right not to explain the source of the money which had been deposited in his accounts, arguing that the constitution gives him that right.

He further argued that Muluzi’s assets could generate more money than the amount of cash the state accuses the former president of stealing.

Chokhoto mentioned several assets including Ntaja Tradings and Chitsime Drilling Company that belonged to the former president’s first wife Annie Muluzi.

Speaking in an interview with Malawi24, ACB deputy director Reyneck Matemba said Muluzi was arrested because he failed to provide an explanation about the money in his account.

“When a person has been asked questions you are supposed to answer, and the accused failed to answer and this brought suspicion and our laws states that if a person fails to explain about his assets he can be dragged to court, those laws were not made by ACB neither the witness,” said Matemba.

Matemba added that ACB will push for justice to prevail in the case.

Meanwhile High court Judge MacLean Kamwambe has adjourned the case to Friday 15.

 

Advertisement

297 Comments

 1. adaononga Boma okha akuluwa mmalo momanga dziko bwino bwino dyera lidawaongetsa dziko mdziko lilimmanja mwa ena pano bweza udF ikadalamulirabe ngati ANC ku south africa adalowera limodzi mdziko mchaka cha1994 koma ANC ikulamulirabe kumalawi UDF idatuluka mmboma mmalo mosapatsila bwino mkululuyu mpira lero DPP,PP and once again DPP. palibeso Fungo loti UDF ingabwerele m’boma never adaononga okha njomba kugolo UDF tinkaikonda koma akuluwa adaononga mmalo momanga adaimasula (shame)

 2. ngati pali munthu amene amandinyasa pa dziko ndikamuona ndi bakili,,,fiti yotheratu ngat uyu sinayionepo kupha anthu much bwanawa

 3. ngati pali munthu amene amandinyasa pa dziko ndikamuona ndi bakili,,,fiti yotheratu ngat uyu sinayionepo kupha anthu much bwanawa

 4. Zopusa basi mwasowa nkhani osamapanga zoti mukweze dziko apa koma kumumanga munthu kwachani anthu mukupondereza dziko ndiinu ndiye umasuke poyankhula osati uzikhala ngati uli ndimalirime awiri chimutu

 5. Zopusa basi mwasowa nkhani osamapanga zoti mukweze dziko apa koma kumumanga munthu kwachani anthu mukupondereza dziko ndiinu ndiye umasuke poyankhula osati uzikhala ngati uli ndimalirime awiri chimutu

 6. WAKE UP MALAWIANS! Palibe nkhani apa, ndipo palibe amene angamangidwe. Peter ndi Tcheya alilimodzi izi ndizopangana, eniake akudziwa chimene akupanga. Ndi ndale izi, Peter akungofuna kupanga clear/kuthetsa mlandu wa atcheya, believe me mapeto ankhaniyi Muluzi adzapezeka osalakwa ndikukhala mfulu. Zowawa ndizakuti boma likupanga mwadala zimenezi pamene dziko lino lilipavuto lalukulu lanjala ndilazachuma, apa awononga ndalama zambiri zimene akadathandizira osauka panthawi yovutayi. Ife amalawi mkumangonyozana kutukwana anzathu chifukwa chankhani imeneyi zoona? no no no, tiyeni tizidekha ndikuonetsetsa amalawi, tiyeni tizikondana amalawi, tisalore kumadana chifukwa cha andalewa. Anthuwa onsewa ndiamodzi amadziwana amachezela amadyera limodzi, zinazzi amapanga kungotitseka mmaso kuti ife tizidana.

 7. Kodi ndichani a Malawi mukutichitisa manyanzi acheya mukulimbana nayo wo ndiosalakwa padusa zakazingati sopani chichokereni pampando olamuliziko zakazosezi munalikt anthu opanda zeru inu mukulibana ndizithu za ziiiiii mumalo mothandiza anthu amene akuvutika ziko mwalilowesa chipwilikiti anthu opanda maganizo

 8. kungofuna pofelapotu a peter muthalikawa mene anachunila achimwene awo….kungokumbutsana oona zandale anati peter ndi joyce banda ndiamene anaba ndalama zambli …posatila ma million anapezeka kuchipinda kwa bingu anangawana ndipo peter sangamange joyce …..leave kuchiteketa alone guys

 9. it looks like chidani chilipo kubanja la Atcheya ndi kwa muthalika coz bingu was the first to arrectd him now is peter wo wont to finish what his brother was statd

 10. it looks like chidani chilipo kubanja la Atcheya ndi kwa muthalika coz bingu was the first to arrectd him now is peter wo wont to finish what his brother was statd

 11. Tikadayenela kumupasa ulemu wake ndi amene adabweletsa ma pgunzilo a ulele aku primary kumuchititsa aliyense kusukusula ndikumaona kunja kuwala inu a Dpp 1999 chipani chanu chidali ndi mavot 5 dziko lonse pano adakutolan ndikusoketsa ndikumaonetsa kwa anthu ali nsalu iyi ndiyolimba ngakhale yatha pano ndi mwayamba kumunyela manja Peter machende ako galu iwe milomo yaikuyo ngat ma bampala a galimoto za kwa manje

 12. Tikadayenela kumupasa ulemu wake ndi amene adabweletsa ma pgunzilo a ulele aku primary kumuchititsa aliyense kusukusula ndikumaona kunja kuwala inu a Dpp 1999 chipani chanu chidali ndi mavot 5 dziko lonse pano adakutolan ndikusoketsa ndikumaonetsa kwa anthu ali nsalu iyi ndiyolimba ngakhale yatha pano ndi mwayamba kumunyela manja Peter machende ako galu iwe milomo yaikuyo ngat ma bampala a galimoto za kwa manje

 13. aMalawi timafulumiza kuyiwala zabwino………Munthu woyiwala zomwe anachita Muluzi ndi galu mbuzi……..mmalo momupatsa ulemu basi muti ndiwakuba agalu inu……..

 14. aMalawi timafulumiza kuyiwala zabwino………Munthu woyiwala zomwe anachita Muluzi ndi galu mbuzi……..mmalo momupatsa ulemu basi muti ndiwakuba agalu inu……..

 15. The best way is for him to prove them wrong not favours if he didn’t still our let him prove no matter how little or long it might take but he is just a suspect.

 16. Muzitsata history anthuni matipate adayamba ndi madala a Chihana ndi a mipingo osati Bakili wanuyo, wadapeza zothaitha kapoloma uyo. Wadaba ndalama za chipatala chachikulu cha pa Kameza, zochokera kwa Gadafi.

 17. Amalawi tili ndi vuto sititha kusiyanisa pakati pa malamulo ndi ulamulilo,, Bakili anali olamula koma anaphwanya malamulo nkuwona lelo izi zikuchitika,, kodi anzanga mukufuna mutanthuze kuti Olemela samalakwa?? Ndende anamangila osowafe?? Dzuka Malawi

 18. Ichi Ncibwana Chaambikachi.Atamangidwa Mwana Wake Sipadatenge Thawi Zazikulu Zidachitika Kulili Iyeyo Bwa?Bliv Me China Coopsa Chichitikaso.

 19. Kodi iwe michael thupa a Maluziyo anakaba kwa mako kupusa mwana wa huleee iwe stupid mbava kusiya yomwe ikulamulayi, K92bn. yija ankagawana malemu champwafu uja mbuzi

 20. km mukamamanga muzilingalila kaye ndiku ganiza kt tikumangai ndilevo ya2 mukachita chibwana wina akufa osa dwala akapezeka akuikidwa ku ndata komwe kuli wakulu. nde ofunika kusamala ameneu bwezi wafa kale kom zinalephela inadusa thawi yake ndi big kahh ameneu munyela muone

 21. Inu mukuti wapanga zazikuli ziti ngati kuli mbava yayikulu nde Bakili munthu oti amati akabweleka ndalama ku ma Bank amayhka ku buku lake panali zeru pamenepa koma mtamati Kamuzu ndikhoza kuvomelako chifukwa amati kubweleka ndalama mkupangila zinthu mdziko ndipo mpaka pano tikanaziwona ndipo palibe chomwe munganene kuti Kamuzu anagulitsa katundu waboma palibe Olo Agogo anu mwafuse zakamuzu akuwuzani bwinobwino

 22. Afufuzidwe basi ngati anaba lamulo ligwire ntchito Bible limanena kuti usabe nde ngati akuluwa anatalikadi dzanja nthawi ankalamulira ija basi zidziwike basi eeeeeetu eeeeeetu!!!

 23. i am die hard of DPP.but i luv a chair u know wy? chair wayenera kulandira ulemu.1.samasungira mangawa 2 salimbana ndi munthu 3 amakhululuka 1-9 mukuziwa nokha.lamulo apa limverepo chifundo.mkaz adathawa ujanso amukoke abwere kuno

 24. ndiye kut akuphweka kumangidwa nd atcheya wa ndalama mukukamba apazi ndi zapakathawi ili nsalu bwez tikut tinasokesa nanga nsalu yang’ambidwa leloyi ndiye mupita nayo lit kwa telala sindikuthandauza kwa ikila atcheya ku mbuyo mayaz komano penanso ife nzika komanso kutengela umunthu atcheya ndalamazo amabadi koma mobisa that min amapeleka ulemu kwa amalawi nanga awa anaba moonekelawa modelela amalawife potiona umbuli nd kusazindikilawa muwakwenya lit u can c now tcheya z fighting 4 his lyf ndiye mukumumanganso mukuganiza mopelewela pomulanda keza paja panakwanila tiyeni tione kaye #cash#gate tione kut atiuza zotani dzuka malawi dzuka sinthawi yokumba pamwala kusiya pa dothi kut tipeze madzi let’s think wisely b4 we go n usamunda ozipasa tokha

 25. Koma kungomanga achikulirewa Malawi yembekezera kuwona zakuda am oversees but dis is the fact Malawi lack of respect to the earlder who fight for democracy like Muluzi n never never get apresident like Bakili.

 26. Koma kungomanga achikulirewa Malawi yembekezera kuwona zakuda am oversees but dis is the fact Malawi lack of respect to the earlder who fight for democracy like Muluzi n never never get apresident like Bakili.

 27. Koma kungomanga achikulirewa Malawi yembekezera kuwona zakuda am oversees but dis is the fact Malawi lack of respect to the earlder who fight for democracy like Muluzi n never never get apresident like Bakili.

  1. Tichotse malamulo tiziyendera zamanyi zakozo? Ngati tizitelo,chuma cha malawi chikhale motani? Kaganizidwe kopusa. Bakili timamkonda,Jb chimozimozi,koma nzopusa kt anthu amenewa alakwila malamulo ndiye wina aziyankhula zopusa,malamulowo tsono ankapangilidwanji?

  2. Tichotse malamulo tiziyendera zamanyi zakozo? Ngati tizitelo,chuma cha malawi chikhale motani? Kaganizidwe kopusa. Bakili timamkonda,Jb chimozimozi,koma nzopusa kt anthu amenewa alakwila malamulo ndiye wina aziyankhula zopusa,malamulowo tsono ankapangilidwanji?

 28. ngati pali munthu woipa pandale,pamalawi pano,ndi ameneyu..amandiwawitsa mutu,ndale zapaubale zinalowa ndi munthu wake ameneyu,..mmalo moti akadalowa a Malewezi,anaika Bingu,ati ugaye,nkumaganiza kt angomukankhila uko Binguyo,cholinga mwana wake (atupele) ayende moyera,mwamwawi Bingu adali wopenya,eeee,anamuchangamutsa. Ndiye mtima womwewo,vairas yagwira aliyese,ndi uyu lero Pitala,komaso jb pano akupanga zamwana wake.

 29. ngati pali munthu woipa pandale,pamalawi pano,ndi ameneyu..amandiwawitsa mutu,ndale zapaubale zinalowa ndi munthu wake ameneyu,..mmalo moti akadalowa a Malewezi,anaika Bingu,ati ugaye,nkumaganiza kt angomukankhila uko Binguyo,cholinga mwana wake (atupele) ayende moyera,mwamwawi Bingu adali wopenya,eeee,anamuchangamutsa. Ndiye mtima womwewo,vairas yagwira aliyese,ndi uyu lero Pitala,komaso jb pano akupanga zamwana wake.

 30. ngati pali munthu woipa pandale,pamalawi pano,ndi ameneyu..amandiwawitsa mutu,ndale zapaubale zinalowa ndi munthu wake ameneyu,..mmalo moti akadalowa a Malewezi,anaika Bingu,ati ugaye,nkumaganiza kt angomukankhila uko Binguyo,cholinga mwana wake (atupele) ayende moyera,mwamwawi Bingu adali wopenya,eeee,anamuchangamutsa. Ndiye mtima womwewo,vairas yagwira aliyese,ndi uyu lero Pitala,komaso jb pano akupanga zamwana wake.

 31. AMUTHARIKA KODI MUKAMANGA ATCHEYA NDIYE CHUMA CHA MALAWI CHIYENDA BWINO
  .MUSIYENI TCHEYA NDI MFUMU OSATI INU CHITSILU CHA KWA AMERICA OSADZIWA MAVUTO WA AMALAWI

 32. AMUTHARIKA KODI MUKAMANGA ATCHEYA NDIYE CHUMA CHA MALAWI CHIYENDA BWINO
  .MUSIYENI TCHEYA NDI MFUMU OSATI INU CHITSILU CHA KWA AMERICA OSADZIWA MAVUTO WA AMALAWI

 33. AMUTHARIKA KODI MUKAMANGA ATCHEYA NDIYE CHUMA CHA MALAWI CHIYENDA BWINO
  .MUSIYENI TCHEYA NDI MFUMU OSATI INU CHITSILU CHA KWA AMERICA OSADZIWA MAVUTO WA AMALAWI

  1. Simudziwa ndale mmangofulumira kunyoza after all muyenela kumuyamikanso Mutharikayu chifukwa mlandu akuyimbidwa a chair apawu ndiwongofuna kuphimba amalawi kumaso kuchita clear nyasi yomwe ena amainenanena chifukwa ACB ati mapepala amaumboni anasowa komanso mwamumva ati nkutheka mboni zina za nkhaniyi nkutheka zinamwalira.iyi ndi drama chabe apa muzipenya uwu ndi mlandu wa fake.chair ndi mlangizi wa president or kuti mkhalapakati wa zokambirana za mmaiko a SADIC pa za mavote ndizina ndi zina nde angamuluzitse mlandu?

 34. koma ndalama ndisatanad….wrongfully arrest konseko kumva kuwawa kut abweze,while people are dieing no medication no food….chifukwa cha munthu modz shame….amene simudadziwebe dziwan kut dziko la mlw likuvutika chifukwa cha munthu ameneu even khan ya cash get kut mufufuze bwino bwino mupeza kuti alimommo ndipo bakili adakalamulilabe malawi coz president angalowe amamuopa iyeyu (God bless my mother land malawi)

 35. koma ndalama ndisatanad….wrongfully arrest konseko kumva kuwawa kut abweze,while people are dieing no medication no food….chifukwa cha munthu modz shame….amene simudadziwebe dziwan kut dziko la mlw likuvutika chifukwa cha munthu ameneu even khan ya cash get kut mufufuze bwino bwino mupeza kuti alimommo ndipo bakili adakalamulilabe malawi coz president angalowe amamuopa iyeyu (God bless my mother land malawi)

 36. koma ndalama ndisatanad….wrongfully arrest konseko kumva kuwawa kut abweze,while people are dieing no medication no food….chifukwa cha munthu modz shame….amene simudadziwebe dziwan kut dziko la mlw likuvutika chifukwa cha munthu ameneu even khan ya cash get kut mufufuze bwino bwino mupeza kuti alimommo ndipo bakili adakalamulilabe malawi coz president angalowe amamuopa iyeyu (God bless my mother land malawi)

  1. Iweyo ndiwakumachinga bakili wakumachinga unganene zoipa zainuyo?chitsanzo chabwino town yakwanuyo ija kumakongolanso kubalaka koma akut kwao kwa…a president shame! inu ndi ine tiyeni tidzingodya nyalau basi

  2. bvuto laife aMalawi ndikuyiwala zabwino basi……munthu wanzeru sangamanyoze Muluzi anakakhala maiko ena bwenzi akumupatsa ulemu……Evans mwina iweyo unabadwira kuZimbabwe unakabandwira kuMalawi sunakaika komenti yopusa ngati waikayi…….

  3. bvuto laife aMalawi ndikuyiwala zabwino basi……munthu wanzeru sangamanyoze Muluzi anakakhala maiko ena bwenzi akumupatsa ulemu……Evans mwina iweyo unabadwira kuZimbabwe unakabandwira kuMalawi sunakaika komenti yopusa ngati waikayi…….

 37. Chipani cha DPP mwaiwala komwe mwachokera nthawi yomweyi kuti lero tiyi mukumwayo chifukwa cha aBakili anakuikani pa bwalo kuonesa kwa anthu kumbukukokani abingu anali ndani ife tonse tinaziwa abingu kyti ndiophuzira chifukwa cha ABakili , kunali aChilumba aMalewezi koma ndisake mulomwe u asiye kudya mbewa, yimethe ku Ndatha kuja amakumba mbewa pa chulu uja mundifunse ine Moses Mwalamba

 38. Enanu mukungolemba zamatama apa anthu akufuna mfundo chonde tili pa fb enatikukamba za kuchigayo kwazaza kusiya nkhani ili kkkkkkkkkk koma zoona Fiona zosaonedwa chakachini

 39. Osataya ntima gys Bokho ikubwela tikamutenga ife ameneyo komanso alamulanso dzikoli ngati alipowina otsusa izi achite nyooo, sakagona kwawo akadzuzimuka alindiife anyamata

 40. mukusewera game ndi munthu wakhulu pamuluzipo bola mutimange totse koma abakili ayi ngat mukufuna mulamulile bwino zitayeni zimenezo ndanena mwamva’

 41. Pakali pano ndi kubwela kumalawiko mwamangayo ndiye munya muwona komanso ndi msilamu, mukhaulamuwona lne Dereck wa Jassi muyiwona Boko Halamu, mumangonva eeti mimba ngati nganga zophwisilana mun’dima, munyamuwona mukonzekele mabomba mukhaula muphetsa osalakwa muwona anyani inu muzikodzela mukhaula

 42. Kodi mukulimbana ndi bakili mmalo molimbana ndiumbawi omwe ulipou cheya anayendensa bwino dziko chatapu pita

 43. Anthu achuma akumalawi sakuba, thieves ndife osaukafe basi. tikamaenda wapansi usiku apolice amatigwira, akuti rogue and vagabond; tikagone ku rest ujeni, ujeni rest house, amatigwiranso akuti suspected thieves. Olemera akamayenda pagalimoto usiku amawasiya akuti afana odyerera, when the rich people are in the hotel rooms these police officers sapitako akuti leave these ana akumpandas alone. Believe me or not, we’re about to compasate this big crook.

 44. Vuto lili ndi ife a Malawi ndi kuiwala lero Muluzi wasanduka chinyalala koma ndi munthu m,modzi wapanga zazikulu ku Malawi akanakhala maiko ena bwenzi tikumupatsa ulemu waukulu, osadanda Madala Mulungu akuona

 45. Inu musataye nthawi ndi kunyozana apa Muthalika ndi Muluzi akuziwana akufuna apasane u President atenge Atupele zadala zonsezo ndi Agalu awa

 46. hishiiiiii my fantastic atcheyaa we malawians we r tied with stupid news ndani sakuziwa kuti atcheyaa ndi boma pa lokha acha lue at the end we hear zat malawi government compersat achair some millions of kwachaz which iz too bad to poor man rk.each politician r mbala zenizeni.

 47. Panyopanu agalu inu kusauka ndikomwe kukupangisani bcz munthu wandalama salimbana ndizithu zoti mulibe phindu olo mutamumanga bwanji ndalama imeneyo sangabwedze mudzangotaya nthawi basi Ndiye potiso mwasowa zopanga agalu inu

 48. Panyopanu agalu inu kusauka ndikomwe kukupangisani bcz munthu wandalama salimbana ndizithu zoti mulibe phindu olo mutamumanga bwanji ndalama imeneyo sangabwedze mudzangotaya nthawi basi Ndiye potiso mwasowa zopanga agalu inu

 49. Panyopanu agalu inu kusauka ndikomwe kukupangisani bcz munthu wandalama salimbana ndizithu zoti mulibe phindu olo mutamumanga bwanji ndalama imeneyo sangabwedze mudzangotaya nthawi basi Ndiye potiso mwasowa zopanga agalu inu

 50. It’s obvious that Atcheya will be acquitted by the High Court,therefore Government must be ready to compensate him with millions of kwacha sourced from poor Malawians.

 51. It’s obvious that Atcheya will be acquitted by the High Court,therefore Government must be ready to compensate him with millions of kwacha sourced from poor Malawians.

 52. It’s obvious that Atcheya will be acquitted by the High Court,therefore Government must be ready to compensate him with millions of kwacha sourced from poor Malawians.

 53. Poti zanu ndi zimodzi, Bola musapange zoti ndalama za misonkho ya a Malawi zipitilire kumila mmadzi kuti mudzampange compersate munthuyi pa nkhani iyi yotha zaka 10 mudakakamba. Compersationiyo + Ndalama adabazo= Billions and Billions of kwachas sucked from poor Malawians.What will we benefit from this case? But justice must prevail by bringing back the lost money.

 54. Mwangozioneseratu kuti inu ndianthu osaopa mulungu komanso osaopa mulungu .mmalo moti mupangezoti ndalama yathu yakwacha ikwere ,ndikumangila apolice , mdf nyumba zabwino ,maganizo anu chitukuko chomwe muziwa ndikumanga anthubasi asaaaah!

 55. My only prezdent in malawi. ndikukaika ngat pazapezekeso wina. even APM himself amaziwa kut chair ndi dolo. a chalume. osat masewera iyai.

  1. Lady, that’s y I hav put “ MY” I knw that we ar 4rom defferent destntion and politcs bt bliv or nt ther’wil b another prezdent compared 2this Guy……….. kumachangamuka pa town kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

  2. Anayesesa pachiyani? Tisanamizanepo apa. Ngati pali historic president yemwe dziko lapansi linamudziwa popanga transform Malawi ndi Bingu Wa Mutharika kunena mowopa mulungu.

  3. A Benga ndakunyadiran tayamba kumvesesana. coz we can’t talk about Bingu without Bakili, then the history iz incomplete. mukunva pamenepo baba? Chair laid foundation stone for these so called Muthalikas.

  4. If u say we can’t talk about Bingu without Muluzi what do u mean??? U want to tell me kuti Muluzi sankayenera kuchoka?? Wake up gys, Malawi its a democratic state that is why we voted for multparty in 1994. Even him nchawa Muluzi told us that Muthalika was a well educated man than him thats why he choose him to b his presidessor. This is why Muthalikas they r still ruling bcz they r cappable

  5. If u say we can’t talk about Bingu without Muluzi what do u mean??? U want to tell me kuti Muluzi sankayenera kuchoka?? Wake up gys, Malawi its a democratic state that is why we voted for multparty in 1994. Even him nchawa Muluzi told us that Muthalika was a well educated man than him thats why he choose him to b his presidessor. This is why Muthalikas they r still ruling bcz they r cappable

  6. Wanga ameneyi namatetule. Wachitukuko. Oyenda mmaliro. Wachilungamo. Wosekesa anthu kumamva kukoma mpaka kuiwalamavuto

  7. pano mpamachezadi…kikikiki mungonyozana aini wakewo chuma chili phwiii ana awo nkumakondwa,inu nsikidzi zili mbwee mnyumba,.kufa, ana anu osawasiila kanthu heedeee.tiyeni tibaacheza chonchi.

  8. pano mpamachezadi…kikikiki mungonyozana aini wakewo chuma chili phwiii ana awo nkumakondwa,inu nsikidzi zili mbwee mnyumba,.kufa, ana anu osawasiila kanthu heedeee.tiyeni tibaacheza chonchi.

  9. pano mpamachezadi…kikikiki mungonyozana aini wakewo chuma chili phwiii ana awo nkumakondwa,inu nsikidzi zili mbwee mnyumba,.kufa, ana anu osawasiila kanthu heedeee.tiyeni tibaacheza chonchi.

  10. mauwa abingu amkapeza 3votes akanawinira kut????,??chabwino akanasia kulamulira koma bingu paekha sakanatenga bomaa

  11. Inu onse anapanga zabwino pamalawi pano chabe kuti mutsimikiza mapuresident onse ndi madolo gwilani ntchito molimbika mphemphelani molimbika muzadzimikiza.inenso ndimatero poyamba koma pano ndinaleka coz ndinalemela pamalawi pomwepani follow my footstep.

  12. Inu onse anapanga zabwino pamalawi pano chabe kuti mutsimikiza mapuresident onse ndi madolo gwilani ntchito molimbika mphemphelani molimbika muzadzimikiza.inenso ndimatero poyamba koma pano ndinaleka coz ndinalemela pamalawi pomwepani follow my footstep.

 56. Mukanati muziganizila kumene mwachoka kufikila lero bwezi musanapange zimenezo kuti mupezeke pamenepo chifukwa cha iye. Mukanamumanga uyu ali kunoyi ku RSA (KUMAGANIZA POPANGA ZITHU)

 57. Bingu arrested Bakili. APM releases him. What a funny folk. This means arresting a former leader in Malawi is a wastage of taxipayers money. Its all about hatredness with predecesors

 58. 1.7 billion muluzi UDF,92 billion Bingu Dpp,40 billion JB pp.Komanso Dpp kuba chipani cha UDF musiyeni muluzi ndalamazake munamubera kale pobela chipani.

  1. A chair nde kuti chani, mbava yachabechabe ngati imene ija, if he was the first democratically elected president it doesn’t mean that he is immune from prosecution, even this bloody Peter Mutharika thing will also be held to account for his failures.

 59. “Wrongly” is crying to replace “wrongfully. ” “wrongly ” says the two are not identical twins!!! Therefore, use “wrongly” instead of “wrongfully”.

 60. Kodi inu osakankoka mmayi ana thawa uja bwanji.mungooneselatu uchitsilu wanu onse,kuti mukhale boma ndi chifukwa cha amuluzi bingu atamuikapo. Tasiyani zokandana ngati anyani lets fornge ahead

 61. Plz plz musiyeni muluzi. boma la mcp linaononga, boma la dpp lidaononga, boma la pp ndiye iiiiiii boma lilipori likubanso why muluzi?oooooooo ai ai ndithu musatero noooonse ndiokuba palibe wabwino musiyeni muluzi

 62. How can I explain this testimony to the public about a great man who help me out in serious illness I have HIV AID for good 3year and I was almost going to the end of my life due to the way my skin look like all I have in my mind is let me just give up because life is not interesting to me any longer but I just pray for God every day to accept my soul when ever I’m gone lucky to me my kids brother run to me that he found a doctor in the internet who can cure HIV online he help me out on everything, the doctor ask for my details, so he can prepare the herbal medicine for me from his temple after all he ask is done one week later I started getting more stronger my blood start flow normally for 4 to 5 days I start getting Wight before 6 days my body start developing my skin start coming up after 8 days which he told me that i will be completely healed, I went for HIV test and I was tested negative I’m so happy that I can say I’m not a HIV patient if you have HIV/AID or any sickness he can still help you in getting your ex-back to you please contact him via his email: [email protected], or whatsapp him on +2348143143878.

Comments are closed.