Drama : Chande in dilemma!

Advertisement
Jaffalie Chande

Jafali Chande’s move to Mighty Wanderers continues to be riddled with controversy as Big Bullets officials claim they will repay the K2 million the Nomads gave to Chande as his signing on fee.

According to reports, Chande may be heading back to Big Bullets barely a few days after signing a pre contract with rivals Mighty Wanderers.

Jaffalie Chande
Jaffali Chande: Being pulled part by money.

Big Bullets supporters Chairman Stone Mwamadi was quoted by one of the media houses saying Chande will return to Bullets in the coming few days.

However, the player reportedly told Wanderers to find a house for him so that he should relocate from Chilobwe.

Chande moved to Be Forward Wanderers last week as a free agent after his contract talks with Nyasa Big Bullets broke down as the team refused to meet the player’s demands.

In a related development, Jabulani Linje and Luke Milanzi have denied speculation that they will move to Big Bullets in the ongoing transfer window and the two say they are happy at Wanderers.

“I am a Nomads player and I don’t have any plans to move away from this club and am happy at Wanderers,” said Linje.

Advertisement

261 Comments

 1. Kelvin Moyo analankhula ekha to mbc sports reporter and i do have the recording of the conversation. Ananenakuti Chande wasankha ekha kupita ku wanderers and we have no problem ife tavomereza and sitikudandaula ndipo we are wishing him all the best. Ndiye lero mukuti chani? A Bullets act wisely dn’t be like educated savages pliz.

 2. Kelvin Moyo analankhula ekha with mbc sports reporter and i do have the recording of the conversation. Ananenakuti Chande wasankha ekha kupita ku wanderers and we have no problem ife tavomereza and sitikudandaula ndipo we are wishing him all the best. Ndiye lero mukuti chani? A Bullets act wisely dn’t be like educated savages pliz.

 3. mbuzi za noma…ask victor limbani,Peter pindani kuti akumenya zotani pano ? bullets imatchukitsa player ….tikuonani ,chande si bullets ,chukepo si bullets sindikunyoza koma musatikwane nawo awa atha kupita ….mamuna sathawa amakhala pompo ndikumenya nkhondo pompo …inunso a kanyuzi aka ndakupilira kokwana ..koma lero lokha nditsuke mkamwa…panyo panu ndithu ndi noma yanuyo

 4. Anoma nkhalani ndi manyazi maule ndipa ntunda chaka chino tikumwanso wamkaka sitimadalira puleya modzi mudziwe chimenecho maule woyeeeee

 5. Kkkkkkkkkkkkkkk kuauction kappena kuti(return to grower)RTG awadi nga burley eti sadziwa kagulitsidwe ka player anazolowera fodya.

 6. READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].
  Truthfully, i was tested HIV + positive for the past 8 years. I keep on managing the drugs i usually purchase from the health care agency to keep me healthy and strengthen, i tried all i can to make this disease leave me alone, but unfortunately, it keep on eating up my life. So last Two Months i came in contact with a lively article on the internet on how this Powerful Herb Healer get her well and healed. So as a patient i knew this will took my life one day, and i need to live with other friends and relatives too. So i copied out the Dr Collins the herbal healer’s contact and I contacted him immediately, in a little while he mail me back that i was welcome to his Herbal Home whereby all what i seek for are granted. I was please at that time. And i continue with him, he took some few details from me and told me that he shall get back to me as soon as he is through with my work. I was very happy as heard that from him, as i was just coming from my friends house, Dr Collins called me to go for checkup in the hospital and see his marvelous work that it is now HIV negative, i was very glad to hear that from him, so quickly rush down to the nearest hospital to found out, only to hear from my hospital doctor called Browning Lewis that i am now HIV NEGATIVE. I jump up at him with the a test note, he ask me how does it happen and i reside to him all i went through with Dr Collins. I am now glad, so i am a gentle type of person that need to share this testimonies to everyone who seek for healing, because once you get calm and quiet, so the disease get to finish your life off. So i will advice you contact him today for your healing at the above details: Email ID: [email protected] or you can also add him up on whataspp +2349036950737. CONTACT HIM NOW TO SAVE YOUR LIFE AND DOCTOR ALSO CURE ALL KIND OF DISEASE AND SICKNESS: [email protected] AS HE IS SO POWERFUL AND HELPFUL TO ALL THAT HAVE THIS SICKNESS

 7. READ MY STORY. ON HOW I GOT MY HIV CURED].

 8. Mugwila Chikolopa Mmene Mukulimbana Ndi Chande Chiwukeponso Akupita Mukalimbana Ndi Noma Ikulizani Musiyeni Chande Wapita Kwa Aluya Anzake Noma Woyeeeeeeeee

 9. Eeeee andudu bullets mitu yazungulila.mwina ndichiyambi chamisala basi.tipange limodzilimodzi tiwatengele ku zomba.

 10. Amene amayendetsa mpila kumalawi kuno ndi anthu adyela kwambil….

 11. Akhale konko asabwere. With or without Chande Nyerere 4 life. Wanderers amayi ndi abambo ndi mtunda wina kuchitekete. Abwerere kwa phokosoko kwathu kunyerere bata ndi mtendere! Umodzi, kumvera, kukhulupilika ndi kusunga mwambo.

 12. Akhale konko asabwere. With or without Chande Nyerere 4 life. Wanderers amayi ndi abambo ndi mtunda wina kuchitekete. Abwerere kwa phokosoko kwathu kunyerere bata ndi mtendere! Umodzi, kumvera, kukhulupilika ndi kusunga mwambo.

 13. Kupupwa kwa bullets nde kumenko malamulo afifa mumawdziwa inu?? Tsani kaye malamulo den mudzipanga bwino zanuzo nkhan iyi yatikwana chande wasainawasaina kunoma n no repay accdng 2 fifaz act musova kampopi

 14. It will be the first time to see such kind of transfer happens since i started following futball for long if happens obviously our rules are not followed and if our leaders allowing it to happen it will be very abomination to all who knows extremely well futball a nbb panga zinthu mozindikira

  1. Phiri Osalimbana Nawo abullets ndi a chamba pajatu, mitu sikugwira nanga kuluza ma friendly awiri motsatana? Noma forever

 15. Koma mma Radio mu mukumvela nkhani za make well, chande ndamene akufuna kubwelela ku bullets yekha, osati kuti bullets ndi imene ya mkakamila ayi, koma team ya bullets yati, iye ali olandilidw ku team yi, koma 2Million yomwe adampasa ngati signing fee idzabwezedw ku noma ngati signing fee ya bullets, nangati simudamvele pa Radio ka audio kake Ndili naka nditha kuku tumizilani pa what’s app, bola kungoyika nambala yanuyo

  1. Chandeyo ndi kape heve. Iye angamafune 3 mitre ku NBB pomwe kwinako akukalandira 2 mitre pali nzeru pamenepo? Kufuna kuikolora team kumeneko? Kwaineyo ndibwino apite baasi asamazimve sugar yekha mapeto ake angotis

  2. Chandeyo ndi kape heve. Iye angamafune 3 mitre ku NBB pomwe kwinako akukalandira 2 mitre pali nzeru pamenepo? Kufuna kuikolora team kumeneko? Kwaineyo ndibwino apite baasi asamazimve sugar yekha mapeto ake angotis

  3. I think everyone got the audio, iwe amene u kuti bodza we uwelenge ma news pepa apa31pano, ife chandeyo timayankhula naye daily pa foni, ukhalila yomweyo BP izakwela Galu iwe

 16. Kkkkkkkkk Akuluakulu Oyendesa Team ya New Bata Bullets (NBB) Mitu Yazunguliraaaaaa!!!!eeeeetiii!!!. kkkkkkk Marilo akatuluka nyumba atuluka baasii Samabwerela kkkkkk kubwelela amakhala Malauro. ndiye inu boolani muzingolira Mwakachetechete kwinaku tikukupepesani Limodzilimodzi. Chande Ndi Wanoma komaso pambali posewera iyeso ndi Saporter mapeto wa Noma ndiye apa!! Musolver kkkkk.

 17. Ena mukanditsutsa ndikanena ine talakwa ngati panali vuto ndimwana wathu bwanji kulankhula naye? Ngati inu mukuyendetsa bullets lero simusamala news 24 yomwe idzalemba zainu.Two games yaswera kuno ku LL pepani bola, fusani agogo Anasimba kapena Akasito.Ntchito ilipo, wamkaka akhalapo koma kulimba kwabwino kukhalapo.

 18. Ine Chande Akangopita Bas Sindidzakhalanso Suporter Wa Team Ili Yonse! Kod Ma Official Mwasuta Tomtom Kod? Mukuona Ngat Zienda? Chande, Msowoya, Tilimbad Sesion Ino? Mukangoelekeza Kulola Kut Apite Ku Manoma Ine Wautali Khalan Nazon Zi Ma Club Anuo? National Team Ndikhumudwe, Club nso? Ndikuopa Kufa Ndi Bp

 19. Haha..chande nd mwana wa mnzeru,iweyo wakuuza zot ali mu dilema? I hop no..nzeru ulbe ndakuona,.#blue

 20. Kkkkk!!koma ndudu bullets yapenga basi,kodi mau akuti once goods purches ar not reternable simunawamve.ife chande tagula sitinabe ndipo sitikubwezerani mukasume kulikonse!!

 21. Kkkkk!!koma ndudu bullets yapenga basi,kodi mau akuti once goods purches ar not reternable simunawamve.ife chande tagula sitinabe ndipo sitikubwezerani mukasume kulikonse!!

 22. Kkkkk!!koma ndudu bullets yapenga basi,kodi mau akuti once goods purches ar not reternable simunawamve.ife chande tagula sitinabe ndipo sitikubwezerani mukasume kulikonse!!

  1. Owo? Mukuona Ngat Zitheka Zimenezo? Iwe Ukut Guds Once Purchased Are Not Returnerble? Kod Chande Ndi Goods? Xul Yake Iti? Kkkkkkk Chande Ndiwathu Basi! Wamva Ngat Zakubowa Kakolope Mu Indian Ocean usovenge Kkkkkkkkkkkkk

  2. kma ku NOMA kuli mbuli zedi mpaka kulephera kusiyanitsa katundu ndi mu2??? Kkkkk bax smunachedwe pitani ku xul ya kwacha mukachotse umbuli

  3. Ha!ha!ha!ophunziranu bwanji zikukanikani kuyendetsa bwino team kumangolimbirana maudindo cholinga muziba ndalama,kwaife2 zathu zinaenda bwino mpake ma player angobwera okha kuzatumikira team inu muzichedwa mkulimbirana mipando coach ndi uja mwayamba kumuloza zala katsala kamodzi pa 9 pano tikakumenyani muzangomuchotsera2 eish!!

 23. Madness,
  at first place why you had to take Sulumba from wanderers? If Bullets sinatenge Sulumba from wanderers do you think wanderers ikadatenga Chande from bullets? I guess NO! Its a tit fo tat game, NKHONYA YOBWEZERA KUWAWA.
  komanso UKAZITOSA ZIKATULUKA USATHAWE. Success its not all about money. Mwalilira ku utsi coz of kusalingalira mozama. Those are kicks of a dying horse, forget Chande, do not cry on over spilt milk…..
  MADZI AKATAYIKA SAOLEKA!
  next time think wise

 24. Madness,

 25. Madness,

 26. In modern football is that possible? Do Fifa rules allow such transactions, I think what Bullets should do is to buy back the player from Wanderers. Apatu agenda katawuluka

 27. In modern football is that possible? Do Fifa rules allow such transactions, I think what Bullets should do is to buy back the player from Wanderers. Apatu agenda katawuluka

 28. In modern football is that possible? Do Fifa rules allow such transactions, I think what Bullets should do is to buy back the player from Wanderers. Apatu agenda katawuluka

 29. Olembanunso pena pake ndinu mbuli{walemba articleyi} when posting try to refer article with rule’s an regulations of football transfer. Umbuli wachukuka taxt me ndikupaseni Malamulo a mpira

 30. Olembanunso pena pake ndinu mbuli{walemba articleyi} when posting try to refer article with rule’s an regulations of football transfer. Umbuli wachukuka taxt me ndikupaseni Malamulo a mpira

 31. Olembanunso pena pake ndinu mbuli{walemba articleyi} when posting try to refer article with rule’s an regulations of football transfer. Umbuli wachukuka taxt me ndikupaseni Malamulo a mpira

 32. Hahahahahaha chavuta ndi chizungu cha pre contract which z b4 nde ngati anoma nda bullets mukukanganirana prayer anima simukuti mwamugula nde ngati Ali wanu pangani terminate contract yake muwalipire a bullets kuti zoxezi muthane nazo khani mose mwayambira chande chande hahahahahahha muyang’ane ma dictionary anu mwina mkumvako meaning ya pre not post b4 end after

 33. I Am Happy Tht He Has Realised Tht He Made A Wrong Decision. Welcome Back

 34. kanundu wakupwetekani eti? mmesa mmamutukwana chande lero mwamufunaso?Anthu openga inu.kodi mukumamikisa ndi chamba mukamasuta? mxiiIiiiiii

 35. please can anyone wth full knowledge identify the meaning of contract & pre contract ?? And what z de different ? Let chande go de soccer lovers tikusowa zolemba kumangokhalira nkhan yake yomweyi yachandeyi basiii aaaaaaa inuu

 36. kkkkkk mwana uyu ndiwanzeru kwabasi sungasiye your mother team. Nyasa akugulirani magalimoti pa loan ndalama mukulandira nzotheka basi

 37. Palibe any dillema apa,wasaina wasaina basi,palibenso kubwelera m’mbuyo,angakwanitse kuigula contract imene anasainayo #andudu bullets?

 38. komatu bullets zakuvutani ine ndinakufunsani kuti kodi akadakhala kuti mukufuna kumugula ku team ina ndalama yake yomugulila iye mukanamugula zingati nde pano mwaona kuti zinthu zikuvuta sopano bwanji kodi inu simutha kugonja bwanji?

 39. Ubwino wake tonse tikulemba ngati sitimadzitstanso za ma contract coz palibe wanena kuti precontract imatanthawuza chani so tiyeni tidzingoyang’ana. Ndawonako David De Gae akulephera kupita ku Real Maldrid dzuwa likuswa mtengo

 40. Be calm Nomas Camp,Chande is our player,komaxo ngati mwini wake asakuifuna teamyo muchitanji kumukakamiza,tiyine tidikire contract yake ingotha mu august,anye nayo akampopi fc

  1. Headline:chande in dilemma not BB in dilemma-the player himself hs made a u-turn..dnt 4get dat u signed the player wthiout the consent of BB where r u going to get the clearance?

 41. Mvuto bullets sifuna kugonja komaso mwina umbuli too much,,, kodi nthawi imene Chande amapita ku wanderes kumakasaina contract ma official a bullets a nalikuti??

  1. Noma inali kale ya ma big ngat the mpinganjira brothers hendrex nguli Banda sherry nsuku ndine wa BB koma makosa ana amenewa amasangalasa si ndale koma zampira, pano vomelan kut Bullets ndi akamuna pa malawi pano

  2. Noma inali kale ya ma big ngat the mpinganjira brothers hendrex nguli Banda sherry nsuku ndine wa BB koma makosa ana amenewa amasangalasa si ndale koma zampira, pano vomelan kut Bullets ndi akamuna pa malawi pano

  3. Noma inali kale ya ma big ngat the mpinganjira brothers hendrex nguli Banda sherry nsuku ndine wa BB koma makosa ana amenewa amasangalasa si ndale koma zampira, pano vomelan kut Bullets ndi akamuna pa malawi pano

  1. Klkkkkk ameneyi ali ndi contract ndi bullets not noma kwanuko anasaina pre-contract so kaya #ayaya_fc mmmmmmm kupoila…

  2. Munthu woti ari ndicontract kuteam ina saangasaineso ina , in this case Jafalie has got a contract with Bullets until August so he cannot sign a contract on top of another contract .akukupeperesani ameneyi ,mumuonaso arimured &white sopano pompa,dont take him seriously.

  3. @ #renald mwina wabadw kumen kampopi akupweteka yamba wafufuza kut malamulo amat chan munthu angasaine contract wit tim ina ngat timu yomwe amasewra watsala nayo miyez isanu ndi umodzi mwna sunamve nd@ six months nde taphatikza zikhadabo zakoz uwne kut kwatsala miyez ingat usamangot fwiyefwye ng@ umazitsa uli mbuli yampira ukoooooo kampopiiiiiii

 42. Phuma bvulo lake a Malawi ndizimenezi mwaona2 kaya muona m’mene muchitir ndi uzoba wanuwo

Comments are closed.