Flames draw in borrowed jerseys

Advertisement
Flames

The Flames Malawi have maintained third position in group L of the Afcon 2017 qualifiers after playing out a goalless draw with Guinea in at 28 September  on Friday in a match they used a borrowed jersey after the team misplaced the bag that had their official kits.

Guinea created a number of goal scoring chance in the opening minutes of the first half but the Flames goal minder was equal to the task as he kept on denying the home team from scoring.

Flames
Flames put up a gallant fight in Conakry.

At the other end, Guinea goalkeeper was on holiday as he was hardly troubled by the visitors’ striking force and the first half ended in a goalless draw.

Come second half, both teams came in with fresh ideas as they were in search of goals that would keep their chances of qualifying to next year’s Afcon alive but they failed to find the back of the net.

As the game was going to an end, Malawi could have hit the back of the net through Gabadinho Mhango but he missed the target and the game ended 0-0.

The draw means Malawi have 2 points from 3 matches. The Flames will again face Guinea on Tuesday at Kamuzu Stadium in Blantyre.

In other group L matches, Swaziland played out a 1 all draw with Zimbabwe and they will play the return leg in Zimbabwe next week.

Swaziland are still topping group L with 5 points whereas Zimbabwe are ranked second with the same number of points.

Advertisement

482 Comments

 1. Mmmmmm atolankhani please try to post true stories flames ndi team ya ziko sikalabu yakumuzi ayi. Well done the flames keep it up.

 2. Hello, am so more happy that you got away point no matter what,what you should know is,Frames is one of the most hard worker team in south and east cost of Africa becouse if we look to the support that this team hard from your government is nothing to compare about other Africa teams.lets talk about here our Bafanabana is earning more help from government but we are nothing in soccer we hard Chilumba young boy(Gabadihno)who shows us that where he’s coming indeed there is soccer,Tata Ghambi Robert,we had Makhosi K phiri(chief) while you keep complaining about your team just help them with the smallest help you have dont look how your friend nation is,they do according there are/have.-from South Africa chief official Orlando pilates.

 3. Hello, am so more happy that you got away point no matter what,what you should know is,Frames is one of the most hard worker team in south and east cost of Africa becouse if we look to the support that this team hard from your government is nothing to compare about other Africa teams.lets talk about here our Bafanabana is earning more help from government but we are nothing in soccer we hard Chilumba young boy(Gabadihno)who shows us that where he’s coming indeed there is soccer,Tata Ghambi Robert,we had Makhosi K phiri(chief) while you keep complaining about your team just help them with the smallest help you have dont look how your friend nation is,they do according there are/have.-from South Africa chief official Orlando pilates.

 4. Good Ppo, i feel like zomasowa zikwamazi zikuchulukila…i would love to advise Flames that next time they are travelling they should distribute the Jersey to every player..be it a Set or two…azayike mu ma travelling bag awo a mmanja aja…in this way ma Jersey sadzasowa komanso it wl mean no need to have a Kit Master..

 5. misplaced bag yakit thats y tadrawa.. tinakavala yathu ija ujk tinakadya zimenezi flames ndi dhilu… onyoxa flames ndi kape

 6. chikwama chimantha kusowa kumene sinanga simunakwerepo ndenge nde chomwe mukudziwa inu ndi kunyoza basii koma izizii zimachitika mudzakwerepo ndenge mudzadziwaaaa.Umunthu ndi kuganiza bwino zizikhala patsongolo panu osati kunyozaa kokhakokha

 7. Mmmmmm anene kuti tinayesako timitera, nanga tiphamvu to panga nawo draw tunachoka kuti pamene atailidwa chinthu chofunika kwambiri?

 8. Koma ndimadabwa amalawi enanu ndimaonangati ndi anzelu koma ndaonakuti alibe nzelu bwanji mmakhala mukunyoza zikolokhalalathu?Tikadayenela kupeleka ulemu ku team yathu ndi kuilimbikisa kuti ichite bwino koma mapeto akenso tikuyamba kunyozanso?Ndangoganizani panopa mayiko ambili akunyada ndi mpila ndipo akutukuka chifukwa choti amasapota bwino mopandakunyoza koma amalawi azanga ndima dabwananu kuti ngati mumalephela kusangalasidwa ndimpila kodi china chimene chingasangalase choposa mpila ndichani?Mziko or mukhale nkhondo,njala ndizina mwaizo koma mpila sasiya kusewela chifukwa chani ife ndiye takhalisisa ndimavutowo kuposa maiko enawo?Kwenikweni amalawi tizazukaliti?ngati tikunyoza team yathu chabwino ngati pali aluso ena sangazionesele chifukwa azaopa khunyozedwa.Tiyeni tipangesapoti dziko lathu ndilathu lomwebasi or tinyoze palibe ndingapindule.Akati dziko ndilolemela alemelesa dziko si pulezidenti yekha ayi koma pali athu ena aluso amene amapangisa kuti ndalama zamaiko ena zizipepeka monga or kuti player wagulidwa ndimaiko ena ndalama zake sagwilisa ntchito yekha ayi zimatha kugwila ntchito zinanso zothandiza nziko.Tiasdalile pulezidenti yekha kuti atukule dziko koma tilimbikise anthu aluso kuti lusolawo lizipitapasogolo.Komanso simapuleya okha pali athu amene akupanga mabizinensi awo ena akupangila kumaiko ena, ena amene akugwila ntchito maiko ena anthungati amenewa akusowa chilimbikiso chathu ena ndipamene amanyozanso anveke kodi iwowa akufuna akhalendani.Ndiye zinthu ngatizimenezi zimabwezelesa chitukuko chanziko mbuyo.Komanso ndikupempha bungwe lazamasewelo lakuno kumalawi kuti liziyenda maboma onse ndi mmidzi momwe chifukwa vuto ndiloti mmidzi muli mapuleya oti oziwampila koma amasowakuti ayambila patipoti akungothela momo mulimapuleya oti team yathu atapezekanso mapuleyangati amenewo athakumachita bwino.Makamaka maboma aku mwela amakhala osalidwa kwambili kumbali yazama sewelo maboma amene wa mulinso anthu aluso muyendelenso kuti mukapeze mapuleyaena

 9. Koma ndimadabwa amalawi enanu ndimaonangati ndi anzelu koma ndaonakuti alibe nzelu bwanji mmakhala mukunyoza zikolokhalalathu?Tikadayenela kupeleka ulemu ku team yathu ndi kuilimbikisa kuti ichite bwino koma mapeto akenso tikuyamba kunyozanso?Ndangoganizani panopa mayiko ambili akunyada ndi mpila ndipo akutukuka chifukwa choti amasapota bwino mopandakunyoza koma amalawi azanga ndima dabwananu kuti ngati mumalephela kusangalasidwa ndimpila kodi china chimene chingasangalase choposa mpila ndichani?Mziko or mukhale nkhondo,njala ndizina mwaizo koma mpila sasiya kusewela chifukwa chani ife ndiye takhalisisa ndimavutowo kuposa maiko enawo?Kwenikweni amalawi tizazukaliti?ngati tikunyoza team yathu chabwino ngati pali aluso ena sangazionesele chifukwa azaopa khunyozedwa.Tiyeni tipangesapoti dziko lathu ndilathu lomwebasi or tinyoze palibe ndingapindule.Akati dziko ndilolemela alemelesa dziko si pulezidenti yekha ayi koma pali athu ena aluso amene amapangisa kuti ndalama zamaiko ena zizipepeka monga or kuti player wagulidwa ndimaiko ena ndalama zake sagwilisa ntchito yekha ayi zimatha kugwila ntchito zinanso zothandiza nziko.Tiasdalile pulezidenti yekha kuti atukule dziko koma tilimbikise anthu aluso kuti lusolawo lizipitapasogolo.Komanso simapuleya okha pali athu amene akupanga mabizinensi awo ena akupangila kumaiko ena, ena amene akugwila ntchito maiko ena anthungati amenewa akusowa chilimbikiso chathu ena ndipamene amanyozanso anveke kodi iwowa akufuna akhalendani.Ndiye zinthu ngatizimenezi zimabwezelesa chitukuko chanziko mbuyo.Komanso ndikupempha bungwe lazamasewelo lakuno kumalawi kuti liziyenda maboma onse ndi mmidzi momwe chifukwa vuto ndiloti mmidzi muli mapuleya oti oziwampila koma amasowakuti ayambila patipoti akungothela momo mulimapuleya oti team yathu atapezekanso mapuleyangati amenewo athakumachita bwino.Makamaka maboma aku mwela amakhala osalidwa kwambili kumbali yazama sewelo maboma amene wa mulinso anthu aluso muyendelenso kuti mukapeze mapuleyaena

 10. Misplacing luggage, how? Lack of seriousness. I believe there shld be someone responsible for the team’s wardrobe. Zina zinyanya!

 11. Musasekei it happen to the other team from east africa i thnk from congo, they ended up playing in Bafana Bafana kit but it was a club playing for caf.

 12. haaaaaaaa de whole malawi ku-iwa- la jersey From to dy i am jersey katunduboy no more forgeting Chikwama pamsana basi yeeeeerrreeeeeeepiipipipipip kwaaaas but gud result pa kamuzu tuesday we r winning 2-1koma chonde pa cctv highlights Malawi cant be known osabwerekaso eti flames fireeeeeee miracle money gooooooo

 13. koma malawi penapake,national team kuiwala jersey analakwitsa kwambiri kukubwerekani mukanangomenya choncho mimba pantunda kut mawa mzakumbuke,koma ndikuona ngat vuto linali kukomedwa ndi town komwe ku guinea

 14. If Flames was Beaten with the Comments which were on Certain Radio Station, Plus Fb,
  – Casting Coach.
  – So many Issues.
  You know Them.
  Mtawali was His Departure, Dismissal instant.
  Koma Nyasandians.

 15. kupanga misplace jersey sinkhani good thing is the draw,anapangako misplace madocument a president ka jersey mkachaniso?

 16. mwina anawaopseza kuti mukangoyerekeza kugoletsa tikulandani Jersey ndipo musewera bunobwamuswe ndichifukwa apanga draw tikanatha kuwina ndithu koma osadanda tidzawaonetsa akabwera kwathu kuno

 17. Malawi ndi wabwinobwino koma anthu akewo ndi a tulo tofa nalo mkonono haha hahaha kuiwala chinthu chofunika ngati chimenechi bwanji osaiwala zinthu zinazo kkkkkkkkkkk mbudzi zamano kunsi

 18. Ine monga mtumbuka chomwe ndinganene pamenepa ndingoti”ma officials ghose nivindele va wanthu chifukwa watikhozga soni aseeee mwe”but congrats to the flames for the job well done its not easy kupanga vanthena ivo kwawene”I LOVE THE FLAMES

 19. Indeed FAM is not serious; can a national team borrow a jersey as if it is a team from the remote area. Do you take only one set per trip? Please be civilized dont put us to shame.

 20. How possible was that a national team proudly known as the frames misplacing the jersey then used aborrowed jersey in a big match like that?I’ve never heard this even local football clubs from villages can’t do like this.We’re lucky that we played goaless draw.

 21. hahaha koma malawians!nde mmapita kukatan ku Guineako?tadrowa chfukwa tinavala ma jersey obwereka otherwyz tikanaluza or kuwina!koma nzokhumudwitsa bwanj,achina Gabah,chiukepo nd timu yonseyo osakumbutsana zoona?kkkkk simmafunikanso kupatsidwa jersey,mkanamenya game nd mimba zanu pamtunda waliwali iyaa

  1. Kkkkkk beta nadi asani angusewe bola lo ndi malufu ngawo pa kweru kt aziwe kt kuluwaluwa nkalusu kamampha cha!

 22. Mmmmm! Amalawi kukonda kunyonza dziko
  lanu bwanji? Ngati mumata kusewela mpira mumuuze kotchi wa malawi national team kuti ine ndimata kusewera or kufunsila kumene ntchito yaukotchi

 23. Anthu eleven plus substitutes plus team officials onse osakumbukako eshhhhhhhhhhhh. Oky ndamva bola simunaluze. But next time please try to remember it musazatichitise manyanzi cause once beaten twice shy.

 24. koma mujerse imeneyi Ebola siinatenge mmenemu,please Almighty Lord spare Malawi since we cannot fight against Ebola,pokhapokha mutakhala nafe,ichi chingatheke. Viva Flames for the draw. God will be on our side when we will be seeing off the Guineans @ Kamuzu soccer Saints.

 25. Vuto lathu a malawi sitikonda dziko lathu,koma maiko aeni timawatenga ngati athu mungadyelele chotani kwaeniko kwanu ndi kwanu..Flames forever!!

 26. Ma comment onyoza dziko lathu bwanji?? Tiyeni tikonde dziko lathu, mpira ndimasewelo chabe, tonse sitingapambane, wina kuluza wina kuluza, maiko ena amakondabe timu yawo ngakhale italuza, nanga ife bwanji tikuzinyoza tekha, ndangodusamo siinatyoke nkhwani

 27. mukamqnyoza team ya malawi mumapezapo chan at the end? team ichinyidwe mumanyoza ika drawer mumanyoza ikawina mumaseka nkumati zogwera nde tinene kut ndinu anthu oganiza?kapena mwa kanthawi kochepa tanenaniko dzina la m’bale wanu yemwe anasewerako mpira inu mbuzi zosaganiza,zopanda nzeru,zopanda mzimu komanso zosowa chonena ndi zosayamika mbuzi

 28. I am surprised that Malawians are blaming their team for drawing away against Guinea . welldone flames. (from Zimbabwe)

 29. I am surprised that Malawians are blaming their team for drawing away against Guinea . welldone flames. (from Zimbabwe)

 30. Zonse zili chabe koma nkhani yofunika komanso yopasa chiyembekezo kwa a Malawi okonda ma Flames ndi yoti osewera athu apeza 1 point ku Guinea. Keep it up guys kuti tizamwe wa mkaka pa Kamuzu stadium this coming Tuesday on 29 th March, 2016.

 31. mpaka jersey yobwereka ?mukuchitisa dziko manyazi guys ,drawyo ndiye palibe chonyadira swaziland won against them nothing worth praising apa g

 32. Kkkkk koma manyasa nawonso mpaka kuvala jersey yobweleka,ur nt serious wth football,nxt tym mudzasewera no jersey mimba pantunda basi mukundipangisa manyazi.

 33. Kkkkkk kuzolowela kusewela bare, APM is to blame akuchedwa kukaonana ndi two horns

  1. And where did you borrow this type of jearsey? You mean the whole team plus officals losing a set of jearsey? Thus unheard off. Akanakukanizani

 34. Nde Malawi imeneyo kuiwala unform kukumbukila tablet yokazinjambulira pa fb….timvaso kuti Gine yafika iwo ndege yathawa kokhala kwawo….mxiewwww paka kukangula unform mu shop ndemaleka lungula ya Red bwanji mxiewwww

 35. Nde Malawi imeneyo kuiwala unform kukumbukila tablet yokazinjambulira pa fb….timvaso kuti Gine yafika iwo ndege yathawa kokhala kwawo….mxiewwww paka kukangula unform mu shop ndemaleka lungula ya Red bwanji mxiewwww

 36. Hehehe! That means Guinea was playing against Guinea. There was no Malawi there. It was like a friendly match. No wonder the game ended in a goalless draw. Nonsense!!

 37. Hehehe! That means Guinea was playing against Guinea. There was no Malawi there. It was like a friendly match. No wonder the game ended in a goalless draw. Nonsense!!

 38. well done draw away sichapafupi mwatichotsa manyazi limbikirani guyz osafooka osatopa ife timakunyadirani welcome back home mudzamalizitse tchito

 39. well done draw away sichapafupi mwatichotsa manyazi limbikirani guyz osafooka osatopa ife timakunyadirani welcome back home mudzamalizitse tchito

 40. Sangakumbuke aliyense anali busy pa phone kutenga zithuzi adzizachayinira zibwenzi zawo akabwera ko sing’anga nayenso zazii kuiwala zantchito asewerera jersey yosakhwimira ndithu

 41. Sangakumbuke aliyense anali busy pa phone kutenga zithuzi adzizachayinira zibwenzi zawo akabwera ko sing’anga nayenso zazii kuiwala zantchito asewerera jersey yosakhwimira ndithu

 42. Ndi m’mene ndiyidziwira flames draw kwa away ndi yokwanira imeneyo, chofunika kulimbika ma game otsalawo kti tikhale pabwno.

 43. Kkkkk jersey. Komanso 28september ndingoona cili conse cocopanda mzeru

 44. Am suprised coz 1st people to comment are the ones who seems like they dont care about Malawi,Mother fuckers Leave Malawi alone we will support them with love and passion.

 45. A vivid follower of soccer world over would never get surprised by that. Borrowing jersey has been there since times in footbaling memorial, only that the reasons vary. However, much as we appreciate that, a strong word has to go to our officials that they MUST be attention to detail every time. Dzikomo.

 46. Since you hv accepted bushiri, expect more till you realise that he is wicked

 47. Mpaka Team Yonse Kuiwala Zoti Ili Ndi Jersey!!! Miracle Money. Team Yagulidwa Ndi Man Of World Iyi Not Man Of God. Kaya Muziona Ndi Prophet Wanuyo

 48. Ma misplacements ndi policy ya dpp gvt. Mwayiwala wolendo wa president Mr Ibu popita ku India? Ma misreplacement omwewo.

 49. Kodi osadzasewelera Ku stadium yaku Lilongwe bwanji? Chizapha anthu chi chichiri cho one day muzaona. Muvi mukuuyang’anirawu uzakulowani m’maso.

 50. Ndiye vuto ndi chani inu chiyambireni simunabwereke zinthu za weni muzimva chizungu chikuti after the team misplaced the bag ndiye mumafuna asewele mimba pamtunda

 51. Borrowed or not,the Flames have done something every Malawian should be proud of.A draw in a borrowed jersey it is not a simple task.I pray for a miracle Flames to give us miracle wins.

  1. A Hema,”yayamba bwino” Kuyamba bwino kwake kuti pamenepa? Anyamata anayamba kale kale awa? Ndimayesa umunewu ndi ulendo okatuluka!!! Our neighbours Zimbambwe have 5pts. Do you think that they will just stay phwiii kudikira kuti Malawi iwapitilire? Ngati anatipha pakhomo, you think kwawoko ndiye zikatha bwanji, kukatimalizitsa.
   Flames in a borrowed Jersey? Ziliko!!!!

 52. Kkkk miracle money imatero imabweretsa ma miracles, dikilani lachiwiri azaiwalanso kuti ali ndi game.

 53. ma Nyasa sazakulanso…..51 yrs stil in slumbre….kkkkkkkkk
  the whole squad forgot the bag!!!! hahahahaha….they were busy admiring the structures in Guinea without minding on what they carried along…..kkkkkkk

 54. Bag imeneyo anawabera nthawi imene aliyense anali ndi chidwi ndi matown anzathu kunjako, ndiye where did they borrowed that jersey? Kkkkk! koma kumalawi. If my memory saves me better; pitala anasololedwaponso chikwama. Zotsatira za masewera a mpirazo ndiye palibe chachilendo we are now just used to it.

 55. Bwanji ndiye simumungomenya ndizovala zanu kaya ma jeans kaya ma shirt ndima two dolar anu olo ma pointer anuwo nanga sizimene munazolowera

 56. Kkkkkkkkkkkkkkk inu team mpaka kuiwala jersey????kodi ndiye mukamasanzika m’makwanumo mumati mukupita kt nanga mukatani?????? Chifukwatu sizoona kuti national team ikagwiritse ntchito jersey yobwereka nanga atakupasani yama coulors oti sianu ngiye muziti chani??? Olo team yaing’ono ngati Jomo cosmos sinapangepo chamba mwapanga apachi

 57. basi enanu ma comment anu nthawi zonse onyonza okhaokha muzakula liti, anthu mukugwesa Malawi pansi ndinu c mutha kukaganizako ngati anthu nthawi zonse shame on you, you have to change & build Malawi together

  1. Iweyo Mayeso ndiye ukuganiza modabwitsa kaya! The whole National Team, misplacing a Kit bag? They were intoxicated with miracle money. Tiwapatsa Sportsteacher waku Golong’ozi F.P. School aziwapangira organize. Wina wake anaguliridwa return air ticket plus hefty allowance as Leader of Delegation only to embarrass the nation like this. Malawians deserve an apology from somebody on this.

  2. long as they put an effort & they got a point kwa ine i jst give a token of appreciation coz aliyense amaiwala basi ndi normal no issue

  3. ati akamanyonza ziko lawo lomwe amaona ngati anthu aziwatchula anzelu chonsecho kuli ku pusa ndi kupanda nzeru ndi kusaganiza shameful people

 58. Osangoseka frams apa ,enanu muli apa ndikhalidwe lanu lobwereka angakhale pant yomwe mumavala wazanu or wa brother wanu,nde muzionetsa kuchengera panano pot flames yabwereka ,shame on u ,olo abwereke mesa ndi zamphira anavara nde vuto ndi chani

 59. Inu Ngati Chinasowa Chikwama Cha Munthu Wankulu Ndiye Kajersey Nkachaniso! Ask Him Akuuzani Uti Sidala! Kkkkk

 60. A Malawi tatani nthawi zonse tulo mpaka kuiwala chomwe tili.zokhumudwisa heve how can they misplace bag yacholinga chawo paulendo wawo?

 61. It would be shameful losing in a borrowed jersey. Strangers in football matters become surprised with things they are ignorant about. Borrowing a jersey is not an issue and in he world football this is not the first time. If you think so coz of your ignorance, find out from true football followers and lovers.

  1. ngati zimachitika ndeumbatamawo ena akut chelsea also borrowed ndeumbatamawo, its not out of ignorance bt just accept akapanga mbola ndi mbola bas no matter ndi chelsea or flames

  2. ngati zimachitika ndeumbatamawo ena akut chelsea also borrowed ndeumbatamawo, its not out of ignorance bt just accept akapanga mbola ndi mbola bas no matter ndi chelsea or flames

 62. Yeah it happens even Real madrid in 2010 uefa champion anapanga chimozimozi koma mwayi Denge inabwera kuchokera ku spain kubweretsaso official kits.ndiye kwa ine sindikuonapo vuto

 63. well done my flames jersey yimeneyo mubwerese ku Malawi muzamenyeretso game yina, yanu yasowayo yisiyeni konko chifukwa zikuonetsa kuti ndiyachitaka yimangotiluzitsa ma game

 64. Ndimabhoweka ndi ma Comment onyoza nthawizonse,bwanji ngati inu muli Dolo osamasewela nawo kuti anthu azikukondani,mukanyoza amalawi inu ndiye ndindani agalu inu

  1. Iweyo chunga umafuna tiyamikirepo chiyani pamenepa? If What they have done was not their did in fashion; I think nobody would dare talked like this here.

  2. Ndiye mukanyoza mumapindula cha??ngati pali phindu Nenani nafe tizinyozanawo kuti tingapindule,mwasowo zochita etiii,sakan # yanga ndikupaseni zochita

  3. inu mukulimbana ndi team iwo akasewera zowo zikuyenda inu mwakoti dwiii,osamapita kome muzikawinako bwanji,munantchito inu,olo mutafa mati anu kungolilira kuti adye chipepensocho

  4. waziziwa Joe,akaluza ndiye tiziwathangisatu nanga tizialalatilanso,ndichikondi pandalama chimenecho,ngati atibe avaye uko akakhala nazo ndi m’bale

 65. Well done guys. It is not easy to snatch a point away anywhere in Africa. Whether u used borrowed jerseys or not is immaterial considering that many a times our own “clothes” had been used to our disappointment. Bravo

  1. Ndiye inu anzathu mudayamba kuutsata mpira kalekalenu tatiuzeni kuti chikwama cha ma jersey chidasowa bwanji.Mwinaso mutifotokozere m’mene katundu wa mu ndege amayendera.Zampiratu izi!!

 66. musanyoze team! Musaiwale malawi24 is ful of disturbing news! Disturbing journalist and shit analysation_ post yanuyi ili senseless

 67. kkkkkkkkkkkkkk hhhhhhhhhaaaaakkkaaaa! what ! borrowed jersey ! Misplaced the Jersey bag !I don’t know IF this happened anywhere else in the World ; wina andikumbutseko ; This is disgrace to country ; koma abale a Malawi tikadali mu tulo la 1939 zoona ?eish

  1. Chif K;kumapereka chinsanzo monga [email protected] pamwambapo ;ndati wina andikumbutse ngati zinachitikapo ; inu mukamba za kuyenda ; Nkuti muyenda inu zikuchitika ngati zimene??chimodzi modzinso @Banda Joseph ; kutsata kwa mtundu wanji mufuna inuko ;

  2. Ndimazoba onse anthu more than 30 ngakhale modzi okumbutsa ,ndege kuwuluka pa stadium kusiya mpira kumawonela ndege zamkutu bas.

  3. If u misplaced something u can find it but if u 4gt mmm u can’t win because u don’t 4get only Jersey komaso ndizida zina zambiri

 68. Imeneyo ndiye flames,nthawi zose imachita zithu ngati adzidzimutsidwa.Mwinaso Guinea ndimene iyambe kufika kuno ku Malawi,tiva kuti Flames ndege yawanthawa.

 69. Flames draw in borrowed jerseys

  The Flames Malawi have maintained third position in group L of the Afcon 2017 qualifiers after playing out a goalless draw with Guinea in at 28 September on Friday.

  Was yesterday 28 September???

 70. Kkkkkkkkkkkkkk koma guyz mukutipasa kuyankhula mwamva kodi muyachangamuka liti zitheka bwanji kuiwala jearsy mu ndege kodi osamala ma unifolm uja alikuti atiuze momwe zinakhalila funso nkumati nanga kumuzi amenyela jeasy iti poti iyo yapita nmtundu wanga kodi watani kkkkkkkkkkk

 71. Apa mukundiuza kuti team yathu ili ndi Jerseys imodzi,nanga wina akadzakokedwa kabudula mpaka kung,ambika zidzatha bwanji may Nyasa!!!!!

 72. anavalayi inali yokongola…..koma yathu ya Umbro timavalayi uhm…..ndiyosaoneka bwino kaya anaganiza bwanji ma designer…i dont know…

  1. Ukati Amalawi kupusa what do you mean? Unakwelapo ndege? Si minbus tu.udont hv control over ur luggage…its at the mercy of luggage handlers…cikasowa it takes tym kuti cipezeke…its either u get it or not..it can even take a month..

  2. Iwedi ndiye ndi chitsiru chamunthu that’s y ukumatenga maina aweni kukhala ako mmalo moika dzina lako leni leni izi zikungowonesa kuti ndiwe chizete chamunthu wamva

Comments are closed.