Prisoners escape from Mangochi prison


Prison

PrisonReports reaching Malawi24 show that seven prisoners have today escaped from Mangochi Prison.

According to Mangochi prison officer in charge Jonas Chimoto, the prisoners escaped between wee hours of one to two o’clock on Sunday using a channel that they had dug at the toilet.

Chimoto added that the channel led a way out of the prison and they dug it using an old axe and knife.

The seven escapees are believed to have been led by two notorious criminals who are answering murder charges.

The remaining prisoners said they were afraid to to alert the warders on duty since the escapees threatened to kill the remaining prisoners if they dared to shout.

Meanwhile, the police have launched a manhunt for the inmates.

(MORE TO FOLLOW)

123 thoughts on “Prisoners escape from Mangochi prison”

  1. Sizachilendo ineyo ndili kumalawi mzanga adaba ndalama za aziphunzitsi nthawi imeneyo asanayambe kuwalipira udzera ku bank. Koma atagwidwa adathawako ku mawula in LLZ. Then ndabwera kuno ku RSA anthu adathawaso ku vereeniging preson why? Wakuba nthawi zonse amakhala wa jakapu.

  2. Apo achita bwino kuthawa ngati woba ndalama za boma amathawa iwo angalephere kuthawa or amati munthu wakuda alibe nzeru amagani moopya muja.

  3. Ine chikhalireni sindinayambepo ndanva kuti ndende ya ku nsanje kapena ya ku lunzu kaya ku kasungu kuti akaidi athawa ayi……koma #mangochi basi ndiye sipamatha mwezi athyola-athyolanso……ngat akuona kuti dzaola osangomanga dzina bwanji???……

    1. Ooooo kodi zafika potukwanizana????……bola ndikanakhala kuti ndaponda pakhomo pako kapena kuntchula dzina lako ndikanati wayenera kutero koma apa pokha wandionjeza m’bale wanga…….stop it!!!!!

    2. Ndipo ku Mangochi last month zinagwidwa zigawenga ndipo nkhani itafufuzidwa zidapezka kut asogoleri ake adali anyamata abeni omwewa. Ndiye ndi momwe zachitikiramu we r not surprised,anyamata abeni omwewo ndiomwe akudziwa game imeneyo.

    3. Kkkkkk……….apapa zangoonetseratu kuti atopa ndi ntchito yawo ndiye sikuti adzingokhalira kumangoguba #pelete kuno nooooo. ..,,,,,, zimafunika onse atachotsedwa ……..mwina tione kuti adzikagubila kuti #beni waoyo

    4. Kkkkk ndiye wina adzabwere kudzandimanga ine ndidzamuthamangitsa moti sadzandifunanso……….nanga ngat anthu akungothawako ndiye kuti awonako chiyani???……..mwina sakudya kkkkkkkkkkkk

Comments are closed.

Discover more from Malawi24

Subscribe now to keep reading and get access to the full archive.

Continue reading