Govt warns of heavy fines for thin plastic sellers

Advertisement
Money currency

The Malawi Government through the Ministry of Natural Resources, Energy and Mining says it will continue to impose heavy punishments against manufacturing companies which are making thin plastics.

Spokesperson for the Ministry of Natural Resources, Energy and Mining Sangwani Phiri said some companies are still manufacturing thin plastics despite government banning the plastics.

Money
Fines await thin plastic sellers.

He further added that the ministry’s aim is to end the manufacturing, distribution and selling of thin plastics in the country.

Phiri said the ministry will continue conducting inspections to make sure that companies are not distributing and selling the banned plastics.

Two weeks ago, government, through the Department of Environment and Climate Change Management, fined Poly Pack Limited, OG plastics Limited, Aero Plastic Industries Limited and Anchor Industries limited K1 million each for distributing and selling thin plastic papers.

Phiri however said the ministry has observed that the four companies are now complying with government’s ban on selling and distributing thin plastics.

Advertisement

29 Comments

  1. Muthamangitse kaye China ija munapanganayo ubaleyi coz ndiyomwe imayambitsa kupanga zinthu zosalimba. Ndiye mukuona ngati anthu anu azipita kuti?

  2. Koma sinachichose cha plastic ngati pepala ndilonyasisa muziko koma ngati kuno kujozi china chilichose ndi ndalama bwanji ukonso kumalawi boma litsegule misika ngati imeneyo anthu azitola ndikumakagulisa mwina dziko lizioneka bwino Ngati kuno

    1. Ndiye Ku joniko zimenezo limagulala ndi boma? Mufufuze mupeza kuti ndi ma private companies ndi omwe amagula zinthuzo enanso ndi eniake omwe amapanga zinthuzo ndiye amafuna akazipangenso kawri zizikudalira boma zimenezo,boma siliyenera kupanga business,umenewo ndi mwai wathu kuti nkhaniyo tiyiunike bwino ndikuyamba business imeneyo,kuno ena amagura nsapato za plastic zakutha, ena amagura ma beseni ndi zidebe za plastic zakutha

  3. BWANJI OONONONGA MITENGOWA IE: A KAMPOPI,BALE, CHIKOPA. KAPENA NDINENE KUTI AFODYA??????????????????????? AMENEWA NDIYE NUMBER ONE.BWANJI OSALETSA FODYA?????? TAGANIZILANI: MIKANGALA, MBALAWALA,MPHANDA,PHASO ETC!!!!!!!!! CHONDE CHONDE!!!!!!!

  4. Mavuto alipo ambiri Malawi muno boma likulimbana ndi maplastic kodi mukufuna anthu afe? Kodi zotsatira zake mukudziziwa Malawi muno umphawi ndi osayamba anthu akudalira kugwira ntchito Ku macopany opanga maplastic womwe what astupid government? Kodi chilegedwechi chaonongeka ndi maplastic?

  5. Mavuto alipo ambiri Malawi muno boma likulimbana ndi maplastic kodi mukufuna anthu afe? Kodi zotsatira zake mukudziziwa Malawi muno umphawi ndi osayamba anthu akudalira kugwira ntchito Ku macopany opanga maplastic womwe what astupid government? Kodi chilegedwechi chaonongeka ndi maplastic?

Comments are closed.