An economic expert in the country has asked Malawians to stop blaming government for the economic turmoil that has affected the country.
The expert, Lyton Chithambo, says Malawians need to start working on ways of developing the country and not pointing fingers at President Peter Mutharika.
“We need to realise that the president cannot provide everything for us but we need to come up with ways on how to develop our country,” said Chithambo.
Chithambo also asked Malawians to be patient as government is implementing a zero deficit budget.
“We have been moving at a slow pace but all of us need to help the country to go forward and develop,” he said
He however said that there is time for everything and Malawians must wait for the right time if they want to choose another leader.
54 thoughts on “Malawians urged to stop blaming govt for economic woes”
Comments are closed.

Kodi nawe iwe Lyton Chithambo wabwera kumene mMalawi muno kapena unali mommuno? Ndikangati komwe a Malawi akhala akupeleka malangizo , komanso kulipempha bomalo kuti litsatire izi izi, kapena lisiye izi izi kuti zinthu zikhale bwino? Chifukwa choti panu zawasokonekera, ndiye akuwafuna anthu kuti athandizane kuthetse mavuto , pomwe pa nthawi yomwe amasolola anthu analibe ntchito, Zimvere mtolo. Pajatu mteinje wa ‘Tinkanena’ udakathira mu nsiizi.

khope ngati. ukubiba. unganene. mau. oti tisiye kudzuzula boma. koma. azipanga zopusazo. eti
Okay thank u
Kodi kugwa kwa zachuma ndi chilala olo mwina pena pake panalakwika mwinaso pena palakwika?
A Malawi adikira nthawi yaitali ku utsogoleri wao, koma osaphula kanthu, ndiye pano zafikapa sizoona kuti anthu akulakwa kulira, ndi kudandaula kwao.
Malawi zinthu zinalakwika poyambirira mu 1964, powumiriza m’Malawi aliyense kukhala mlimi, womwe waika usiwa wadzaonene ku anthu ndiponso pa za chuma.
Munthu aliyense anabadwa ndi talent yache yokweza moyo wache ndi wa ena, koma matalent a Malawi ambiri anafera kudzenje.
Lingakhale dziko lanji pansi pano kudalira chabe ma Export aza Agriculture yemwe ikudalira mvula basi? Fodya akhala akuyendetsa chuma cha Malawi kwanthawi yonseyi, nanga bwanji migodi mafakitale zamatransport apanyanja Ilala yeka ndi zamtokoma zingathandize?
Ngakhale mvula igwe bwino bwanji mu Malawi chuma sichidzakwela kaamba kodalira ulimi woka, ndi chitsulo chomwe ukachigule kunja, Galimoto tisanene.
Kodi chizungu chija mumatiphunzitsa pa Agriculture Ubwino wa Crop Enterprises unali wotani?
Nanga pano boma silingapeze nzeru ina yokwezera chuma chake kuthandizana ndi ulimi?
Azamalonda adzayambitsa bwanji malonda pomwe mphamvu ya getsiso ndiyocheperapo?
Sigetsi wa industry mukumuonayo ndiwowunikira mphamvu zache pa Industry growth akuchepelatu,
Atsogoleri onse nzeru zao kuti aike maplan, mitu yao yaima nji,
Mwaphetsa mtundu wa a Malawi omwe ali ponseponse mu Africa, Europe ndi Caribean, kukadzifunira,
Utsogoleri ndi nzeru zoyang’ana patsogolo osati ine ndili ndi ma digili, awo azamaphunziro zakanika zinthu.

Economic expert? are you really an Economic Expert? Wadyandalamazabomakapena? Amenealioyenelakumudzudzulapanyasizimenezindani? Mbuzi
Kkkk ine mpeeeeee pa durban ndikulimbana nditchoto ndikutandixa abaleanga asagone ndinjala