Traffic officer caught demanding bribe

Advertisement
Corrupt Malawi Police Officer demands bribes
Corrupt Malawi Police Officer demands bribes
Busted! Malawi Corrupt Traffic Police Officer demands bribes

Corruption continues to haunt Malawi as a local traffic police officer has been caught on camera receiving a bribe from a white man at an undisclosed roadblock.

The identity of the officer is not yet known, neither is that of the foreigner since the video clip that has gone viral on social network does not reveal their faces.

The 36 second long clip shows a white man sitting on a passenger’s seat while talking to the officer through a fully opened window. Then he gives an amount of K7000 to the law enforcer in exchange for an envelope that is understood to contain documents that can allow the white man to travel without any hindrances.

From the look of things, a person driving the white man does not have a driving licence which forced the traffic to hold them.

“Is this how you pay a bribe in Malawi?” asks the white man, to which the officer responds with a “yes”. Then the Malawian civil servant asks the white man to make sure that a licence is processed for the driver.

The clip has attracted a myriad views from Facebook users. People have slammed the officer for engaging in such an uncalled for act.

Advertisement

217 Comments

  1. Nanga atani boma lakweza mitengo milandu ya mpaseu komanso ku road traffic zochitika zimbiri mbiri.Nalonso ndilakuba. mamember tiyenazoni musasiye.

  2. Boma lipange zotheka a Malawi tidziwe mitengo ya milandu! Osati kumangolota, mkumango charger kuti aziti “Pali zingati?”
    Tizikalipila pokhomela misomkho basi spot fine ithe, Mwina ziphuphu nkuchepa koma osamachedwetsana panseu kuma khala ngati wa traffic ndi bwana chonsecho si bwana nkomwe! Imadya pomwe aimangilila ofcoz koma zinazi is 2 much. A Malawi kumayankhula osamasekelera nzopusa zomwe ai! Mbava zilitho m’madelamu koma iwowo akudzadzana panseu kulimbana ndo pita ku ntchito!

  3. Malawi 24 think b4 posting ur stories dis picture sikuwotsa zomwe mukunenezo abodza ndinu basi mumangoyilonda galimoto kuti mujambule mukuyesa ndife ana eti tapitani ku state house mukajambule msomba zikuluzikulu kaye then we are going to hear u

  4. Salary hike cannot change one’s mindset. If we talk of comfortable government department it’s immigration. People should first know their rights and what they are paying for. One pays for an ordinary passport and bribes the officer to get it within a week? It takes two to tangle. And you pay for an express passport you find the window period has expired you take them to task. It’s your right. My dear country men, work up, don’t allow people to take you for granted. This spirit of Luke worm altitude/humbleness is what is killing us.

  5. Mvuto lake ndilimenelo a Mw 24,mukulemba izi coz ndi white guy kkkkk,koma adakakhala wakuda ngat ine mmmmmmmm bwez kuli ziiiiii.

  6. Apolisi ndi abale athu ponda apolice sibwezi zili bwino….kukugwila speed trap 10pin nde umalandira 35pin/mon kudandaulira akuti bweletsa 35 to me tis not abribe..ndiza pauchibale poti ndife abale ndi apolicewo….DZIWANI KUTI APOLICE NDI ATHU NGATI IFESO SANACHOKELE KUMWAMBA AI CHOSEN AFEW Anango chita mwai.

  7. tatigairen clip yo tu nanga mukungoti seculating on social media aliyense akuti alibe kaya +265882191993 tatiponyeren pa whatsapp

  8. Apa mwanamiza munthu aliyense owerenga bodza lanuli basi. Do u min ojambula ndikamoseko anali nawo mgalimotomo kapena chapatali penapake..nde Mau mwanama kuti amanenedwawo mwawatenga kuti?? If u r confident inaccurate of wat u r saying here nkhope mwakanikiranji kujambula nkukanama zamapepala ngati Maliki!!!!! Despite kuti zuphuphu ziliko bt dis z avoid lie…………………

    1. Ndizoona broz sakunama,hope foniyo anangoitchera m’galimoto momo & ndimava ngati akuti amupangaso kale demote nkulu ameneyu koma he is a good guy kungoti zimangochitika poti nditsoka basi.

    2. Ndizoona broz sakunama,hope foniyo anangoitchera m’galimoto momo & ndimava ngati akuti amupangaso kale demote nkulu ameneyu koma he is a good guy kungoti zimangochitika poti nditsoka basi.

  9. I agree with you Ken Chinangwa. But they are other pig headed strong Malawians who do not understand this. All what they are doing is to judge others comments but here they refuse to comment their innermosts feelings towards this issue. All they need is to blame others points of views on comments.

  10. That white mad had to be arrested… He is the corrupter…. If you take banana to monkey and he ate it , whose fault is it…. Please arrest that white man…. Corps in America ,London , China and Dubia do the same..

  11. Malawi police is the highest corrup police in the world as well as the lowest paid police in the same world,any relationship?

    1. A potent comparison to be sure… but that still does not excuse the officers actions. It should highlight the issue to the government though.

    2. A potent comparison to be sure… but that still does not excuse the officers actions. It should highlight the issue to the government though.

  12. Is the picture showing a Police office recieving bribe (money) or peeping through the window? Is this a video or a still image? Tell people the truth!

  13. nkhani ya ziphuphu tiyeni timusiire mwini wake Mulungu adzaweluza yekha,lero siizi tikulamulidwa ndi munthu oti in true sense sikuti anawina ndi iyeyo ayi.Ndiye tikamakamba za ziphuphu ziri pena paliponse.Ine ndikufuna akanangobwera Ambuye yesu aliwotchepo dzikoli timwazikanepo.

  14. Malawi police is highest corrupt police in the world as well as lowest paid police in the same world,any relationship?

  15. VINDICATED!I hv bn sayng tht we hv 1 of th HIGHLY CORRUPT Polic in th world.They dont care whether ppo see it or not.It is not onl traffc polic tht is corrupt it is almst all th DEPTS of th institution.Thes days th BEST police is MONEY.

  16. plz go ahead let them go ,make corrupshion free sothat our contry can go up .amat mbava ndiyimene mwagwila tiyen naye amenewo kundende basi

  17. palibe khani apa inuuu,,, awa ndi anthu odziwa mabvuto pa malawi., kangachape amalandira., kuopa angakuchedwetse pa ulendo., kukhala sikoma uku.,

  18. Zimakoma kuba, koma ukagidwa, mpamene umaoneka ukape wako wonse. Mmene amachitira a police traffic awo, mmsewo wochokera Nkhatabay kupita ku Mzuzu, amanyasa anthuni. Ine ndakondwa nazo kuti wina wa iwo wapezeka. Mumusewu kuchita kuthinana ngati ngumbi abale in? Minibus kulephera kudutsa bwino.

  19. Atchulidwe dzina ameneyi ndithu ..mukumudziwa bwino lomwe simungangolemba nkhani munthu osamudziwa ..zichitila ubwino amalawi mukatelo……zikomo.

  20. يا جماعه عاااااجل يا جمااااعه لاول مره فيه كروت شحن بجد من موبــــــينيل و فودافـــــــــــون واتصــــــــــــــــــالات ببلاش العرض شغال وبيدي كروت شحن بالفئه والنوع الي تختاره ا العرض لفتره محدوده جدا والي مش مصدق يخش يشوف تعليقات الزوار http://arapmarah.talk4her.com/h104-mganan-new-kro0ooot-sha7n-2016

  21. Pieter Cisale, did you get my point clear? I said World Wide. Re_read my point please. I don’t want obsteperous rumors rising against me in the end that am underrating my country.

  22. Dziko limadana ndi oba pang’ono, oba zambiri amadziwa adya naye zambiri. Ma big fish a cashgate pano sakumveka koma opha anthu chifukwa cha ufiti.

  23. I agree with your statement Gama waku Thyolo. I think some people have just grownup without seeing how tough the Government of the late Kamuzu Nanda was. They just hear stories about Kamuzu.

  24. kamuzu banda anakamba kale kuti matimati mukuwafuna lerowa muzandikumbuka pano nthawi imene ija yafika anthu tikulira palibenso angakwanise kuthesa mavutoawa

  25. Ndeyache buyache.zambiri zinabedwakare Ku statehouse. Bwanji ma big fish sakugwidwa.komaso zammaja mitengoyakw imakhara yabwino pamene ya boma ndiyokwera,pomwendalamazo akabanso anthu andare kuyiwara.anthu akuvutika nzipatala

  26. Kkkkkkk… I kn ze traffic police officer.. works around LL city.. u will find hm most behind zat road passes behind LL hotel.
    Wat a shame.

  27. Komatu penapake mukumadabwitsa. Kodi akati mtolankhani, ntchito ndiyotani? Mukumalimbana ndi atolankhani pa zinthu zii. Koma ku Malawi kokha, nchifukwa chake tikadali kutsalira ku mbuyo mu zinthu zambiri. Kaya ndi umbuli, kaya ndi matenda, kaya ndi chani kaya.

  28. Ndie bvuto ndicani,nkaesa mbuzi imadya apa aimangilila?kodi mumati akakudyelani kutiko?ziphuphu zonse zilimdzikomo ndie chiphuphu chocepa ngati chimenecho muchipezele bvuto?

  29. Inu aMW24 ngati mukufuna kuti asiye mulembe za mavuto awo kuti malipilo awo akwele coz 40grand pamwezi ndiyo chepa lets break it timutenge wapolice kuti akukhala nyumba ya 10pin ameneyu ali ku rular area nanga wa town ndi zingati? Chimanga pano ndi 15pin thumba, ana feez alipile madzi/magesi kuti adye 1to30 abale ku mudzi akudalila iyeyo fertiliza asamale makolo ake 40grand yomweyo MW24 mulembe zoti mavuto awo athesedwe mukaone nyumba zawo ask mkasa ndiye apa mukuona kuipa kwao za mavuto awo simumalemba kusonyeza kuti alibe mavuto sichoncho inuyo ndi amene mungawathandize kuti ma salariez awo akwele powanenela kwa awooo osati zomwe mukunenazi nzopanda nzeru mwamva inu!!!!

    1. Take ur time ucheze naye ndikumufunsa mavuto ake wapolice yo uwll tell me tisamangoyang’ana vuto tiyeni tione chomwe chikubweletsa vutolo ndiye tikonze kuti vutolo lithe

  30. No problem, there is no bribe there that guy gave traffic officer money just for cold drink k1000 only then you are telling me that it’s bribe?
    how much does Mr Muluzi steal?
    and Bingu, job
    and now it’s Peter these people they stealing our money

  31. Kumbukani posachedwapa ma atolankhani ena anapita ku Road Traffic nakapangisa Driving Licence within two days and Malaria Certificate at Queen Elizabeth hospital for a day. They tod the Minister that at RT and Q. E corruption is at a high level. The Minister said ” no evedence” Atolankhani anayeseza kuti umboni ndi omwe tabweretsawu. Nduna “sukwanira” ndiye lero ati chani?

  32. This was a plot. The one taking the camera in this case Mzungu new what he was doing and the poor officer did not know anything. The driver and Mzungu planned to have no license not that they did not have it but to fulfil their agenda. In this case the one giving a bribe also has a case to answer.

    To the author of this article says that their face is not showing and yet we can see it from the clip Itselt if you want to see like we see it on the article

  33. Bribs iz everywhere y chuleyo didnt explain about bribs in europe ? He mustnt go with that vidio clip it must be confiscated .

  34. Some people have great misconceptions. They don’t understand what somebody is narrating them about the current situation in Malawi. Chosamva, adachiphikira mumasamba.

  35. mlaka ananena kale kut wachuma akaba amat zilibe umbon bt the same things when poor man acts will end up in custody y don’t thy focus much on billions gone b4 ( cashgate ) bt busy wth minor stories leaving major ones behind

    1. Lonjezo Bande where’s that name come from if they don’t pay why he ask him that is that how how u pay bribe in malwi

  36. Munthu Wamkuluyo Sanalakwise Ana Ake Akafe Ndi Njala Iye Ali Moyo? Zimenezo Nde Zofunika.Kuuphunzitsi Timati A Teacher Must Be Resourceful. Ngati Zipangizo Zina Palibe Munthu Umayenera Upeze Njira

  37. Munthu Wamkuluyo Sanalakwise Ana Ake Akafe Ndi Njala Iye Ali Moyo? Zimenezo Nde Zofunika.Kuuphunzitsi Timati A Teacher Must Be Resourceful. Ngati Zipangizo Zina Palibe Munthu Umayenera Upeze Njira

  38. Eneless p. Dzuwa, as Iam talking, am no longer in Malawi there, koma kungoti I do comment kumvera chisoni a Malawi anzanga, chifukwa munthawi imene mulimoyo, ndi nthawi yolakwika. Zinthu sizili bwino. I left Malawi, some 4 year ago. Komano, kwanu nkwanu, oro kuyipe sindinganyozerenso. Mawa zikandivuta, ndizabwerera kwathu.

  39. Vuto ndiloti, pali Anthu enafe oti sititha kuchita focus komwe tachokera ndi kumene tikupita kuti zikusiyana bwanji? Ena a ife amene tinawonapo ulamuliro wa Malemu Kamuzu Banda, titha kusiyanitsa kuti Malawi wakale ndi Malawi watsopanoyi, zinthu zili bwanji ngakhale kale lija inali one party system of Government. Lero poti ndi multiparty system of Government, aliyense ali ndi ufulu kuchita zomwe angafune. Komanso, ufulu umene tili nawowu, watibweretsera mavuto adzaoneni.

  40. Kungosamuka amene akuona kuti kumalawi kwaola basi ndi kupita dziko lomwe anamva kuti kulibe mavuto kusiya ndi kumangolirapo yapa!

  41. Inu Azathu Apa Msewu Pitilizani Kulanda Za Mmanja Mumatithandizabe Bola Asakukwidzingeniso Nanu Chifukwa Tikhoza Kufanana Muzikalima Kachewele Ku Madimba Mutatha Plan.

  42. Mike Gama, don’t judge others comments. If you have a comment, you better share it and nobody will judge you. The point is this, during Kamuzu Banda’s rule, did you ever heard about such malpractice taking place in Government? You have to think wise. Some people are good at blaming others comments and I don’t know, why?

  43. This is newsworthy, I support it! ilookfowward for documentaries like the one which happened in Ghana. unless we change from our homes, roads and workplaces to deny bribes and corruption we will remain underdeveloped.

    1. Well Malawi has always been the same I don’t know the Malawi you use to live but corruption has never left the country

  44. You journals also receive bribes not to publish some other stories timadziwa mumati akadya kuti? One ndapeleka bribe mmawa womwewu I have no cof and insurance k2000 ndadutsa pa lumbadzi

  45. Malawi24 mwapangapo izi….mukamaenda munseumu…this department is the most corrupt depart in Malawi….look at some of the cars on the roads and you will understand what i mean……

  46. Mbuzi imadya pomwe aimangilira,mmati akakudyeleni ku chpatala?Ku chipatlanso kulibe chakudya..zikumuwawa akakolope lake MW..Kuli katangale kunjaku osat K7000…uzoba eti mmxiii!!!

  47. A welcome development What is K40,000 salary per month.In addition dont let any vehicle pass through the roadblock without any bribe or else your family may die of hunger.

  48. Ndani anganene kuti sapanga corruption mma office anuwo ndiye mwanyanya bwanji simugwila aku immigration pakuti ngakhale mathanyula wanuyo akuzidziwa zimene zopusa basi

  49. Wachita bhoo ameneyo azungu kuno sikwao en chonde apolisi apamseu ngati mwai wapezeka chitani koma kusamala coz maphon ena ali ndi macamera ambali

  50. Mwaziwa liti zimenezi ife tinazolowela timaziwa kut paliponse tikumane nawo tipeleka ya drink zot ndi corruption mwatero ndinu galimot ngakhale yopanda chilolenzo pa sewu bola cash bas inu mumaona ngat mukuba nokha azanuwa a ngoyang’ana inu mumat akamalawila kutchito ndekut akuikonda ?

  51. …I would rather accept a bride than going to bed on an empty stomach, if you want to fight corruption then you must kill the big fish beneath the ocean.

    1. Salire katangale tidamupeza or nthawi ya kamuzu amati katangale aposa salary the only thing is that it’s no how they pay it in Europe baba

  52. No news here everyone in Malawi even a church rat knows how those in uniform on the roads corrupt are, they can even tell you that they dont have relish at home, all what they know is money exchanging hands! no wonder you have one hundred road checks masquaradinn as blocks yet to in true sense its fund raising for their bellies”kupempha kuposa radio maria” smoke and expose them.

    1. Chilungamo chiyende ngati madzi I once witness a fight amongst two of them fighting after atapondana 20 pin yomwe anaipata pa nseu! they even said katangale aposa malipiro! shame

Comments are closed.