Mutharika fires bodyguard after his ‘fall’

Advertisement
Peter Mutharika

Just days after he fell down, Malawi President Peter Mutharika has axed one of his body guards, Malawi24 has learnt.

The bodyguard, Superintendent Ben Mwaliwa has since been sent to Nthalire Police Station in Mzimba.

Peter Mutharika
Sorry Mr President

According to reports, Mwaliwa received the new role in the just ending week and his demotion is being linked to the fall of the Malawi leader, but police officials have denied.

Close sources have tipped Malawi24 that Mutharika was angry that the bodyguard did not scout the place where he stumbled.

But police officials say the transfer is normal and should not be linked to the recent tumble of the President.

Last week, Mutharika took a fall while trying to plant a tree at Kamuzu Palace.

It is said that after Mutharika had planted a first tree, he had trouble planting a second tree and did a ‘Mugabe’ in full view of the camera.

His fall came amid reports that he had been ill, something the State House has been denying lately.

 

Advertisement

795 Comments

 1. Mukamagwa osaloza chala mzanu!! Akakhala pa Mkhate khoswe amavuta kupha anakakhala munthu wamba!! Ndazapansi pompano izi.

 2. One thing I like on this issue Mutharika is still strong and doing his daily office duties and someone who can’t afford to buy even A pair of suit is busy celebrating that the President should die but the bible is saying that we should honour our leaders no matter what. I think this is why Malawi is a cursed generation ever in Southern Africa

 3. Amalawi anthu amayiko ena aziona mukunyonza mtsogoleri wanu chifukwa chakuti anagwa mmmmm uwu ndi umbuli tamawonani zinkhani za maiko akunja ma coment ake,ngozi ndi ndale mzosiyana koma peter ndi munthu ngati inu kugwa amagwa aliyense bola ali munthu iye si mulungu kuti sangagwe ai eish malawian peaple mmmmm

 4. Even ku Egypt ana a Israel anavutika mu ulamurilo wa pharaoh koma mulungu anapeleka njira 2 deliver the Israelist..shud jst beta die mayb 2 hv peac

 5. Even ku Egypt ana a Israel anavutika mu ulamurilo wa pharaoh koma mulungu anapeleka njira 2 deliver the Israelist..shud jst beta die mayb 2 hv peac

 6. tsoka onyoza kholo lake Pulezident ndi Bambo wadziko lonse komano umbuli uli kuno kwathu ku Malawi tikakhuta kopwetsela mkwa apulezident tsoka Njala kodi lemba limatinji?APM ndindani kuti akagonjetse njala?tsoka,tsoka onyoza kholo.

  1. young lu ndani sanamvepo za mbiri za njala BAIBO ikunena momveka bwino dzulo magetsi/madzi zimavutavuta mumatukwana APM mumafuna azikapopa yekha madzi ku Walkers Felly tsoka onyoza kholo lake.

 7. Kwa muthalika kuli matenda akugwa chocho akuluawo anagwaso ulendo unali omwewo nawoso awasiya dala kuti alape jehova wawakondera

 8. Kwa muthalika kuli matenda akugwa chocho akuluawo anagwaso ulendo unali omwewo nawoso awasiya dala kuti alape jehova wawakondera

 9. Kwa muthalika kuli matenda akugwa chocho akuluawo anagwaso ulendo unali omwewo nawoso awasiya dala kuti alape jehova wawakondera

 10. Why to fire a body guard u don’t have faith in your self fire ur self sir African leaders don’t think u can control everything fear God he is the best ever body guard think about the poor those who need help copy good leaders be friends to those leaders look at ur country Mr be ashamed

 11. Dreamers Training Centre
  (Blantyre Campus)
  (Cambridge A/AS-Level/O-Level & IGCSE)

  Subjects Offered: English-Literature, English-Language,Physics,Chemistry,Economics,Accounting,Biology,Mathematics,Spanish,Portuguese,French,Geography,History,Psychology,Sociology.etc

  Categories: Weekdays, Weekend & Evening Classes.

  For enquiry, contact: 265 884 319 996(whatsapp) OR 265 999 138 103(call).

 12. Mmmmmm……nkhazatu izi. As if you are telling us Kugwa is not normal. That’s so naive of you Mr P. I thought people were wrong taking a meek out of it but now I don’t blame them.

 13. Mmmmmm……nkhazatu izi. As if you are telling us Kugwa is not normal. That’s so naive of you Mr P. I thought people were wrong taking a meek out of it but now I don’t blame them.

 14. PLZ PLZ THERE IS NO PILICE STATION OR POLICE POST OR POLICE UNIT IN MZIMBA BY THE NAME OF THALIRE.BODZA LAYAMBIRA PAMENEPO

 15. Chilima nthawi yako yatsala pang’ono kut ulamulile dziko …mmene zatelemu zayambika….ulowa mchamutu ngat mai joyc banda

 16. mugabe anagwa sanadane ndiwina aliyese anaziwa kt wakula.ndiye musadane body gard mwatopa phavu akukokolan anamaseko ngat mutsutsa mumpatse mimba november tione baby

 17. Kwacha inagwa akusowa oidzutsa,inu kugwa munadzutsidwa nde mukanchotse ntchito okudzutsaniyo?bola munakati sanakudzutseni,kwacha bwanji sikudandaula kuti sikudzutsidwa?

 18. Anthuni muzilondoza nkhani musanakomente remove negative attitude. Bodi gadi amuchosa chieukwa chopanda descipline popeza amalumikizana ndi ma media kumafalisa nkhani yoti President wagwa Which is childish because ndi ngozi yachilengedwe ndipo munthu ndiye okugwayo

 19. Mchifukwa Chani Tataya Chikhalidwe Chathu Tinayamba Bwino Tikumaliza Kuipa Musakhale Ngati Ana Anjoka . Every One Hs A Right To Privacy , Bodyguard Watumizidwa Kukagwira Ntchito Kwina Ali Ndiudindo Osintha Antchito Ake Mufune Musane . Ndangodutsa Sinatchole Nkhwani

 20. Mchifukwa Chani Tataya Chikhalidwe Chathu Tinayamba Bwino Tikumaliza Kuipa Musakhale Ngati Ana Anjoka . Every One Hs A Right To Privacy , Bodyguard Watumizidwa Kukagwira Ntchito Kwina Ali Ndiudindo Osintha Antchito Ake Mufune Musane . Ndangodutsa Sinatchole Nkhwani

 21. Last year Robert Mugabe adangwa koma ngakhale modzi adachotsedwa ntchito, ndiwe ndani to fire someone coz wagwa, kupusa ya!!!! WE DON’T NEED YOU GO TO NTHATA

 22. Last year Robert Mugabe adangwa koma ngakhale modzi adachotsedwa ntchito, ndiwe ndani to fire someone coz wagwa, kupusa ya!!!! WE DON’T NEED YOU GO TO NTHATA

 23. Kungofuna kuongetsa ndalama zaboma munthu ameneyo boma lidzamulipila ndalama zambili if not today z tomorow paja boma siliwina mlandu

 24. Stupid president! Who told him that he won’t fall down? Let us wait n see who will be fired wen he die thats not the reason for someone to lose job in a cheap way

 25. KUMAKHALA NDI UMUNTHU. KODI ATAKHALA MMODZI WA MAKOLO ANU BWEZI MAKUMAPANGA POST NKHANI NGATI IYO PA SOCIAL MEDIA CHONCHI? ZOMVETSA CHISONI. KODI AMALEMBA NKHANIYI NDI WAMOYO? NGATI NDIWE WAMOYO UPEPESE PONYOZETSE MTSIGOLERI WATHU.

 26. mukangosainila ndalama zokuti zizithandizira mathanyula mziko loopa mulungu lino ai ndithu makala yamoto akukudikira ndipo imfa yowawa uilawa chakachi chisathe

 27. Mmalo momalimbana ndi njala ,komaso chimanga chikusowa mwa admarc ,mavenda nawo afika pa k270pr kilo, kodi choncho mutundu wamalawi ungakuvoteleniso pamene pano akugona ndi njala pofunika muganizepo bwino ,ndimuja athu amaganiza zochita upandu okuphani ngati chimwene wako bingu wamutharika .

 28. the body guard deserves being fired, its the duty of any body guard to protect the body he/she guards at all costs from any unncertainity except natural disasters like thunder and lightening, usilikalitu siophweka as others who had never been soldiers think,command siimalakwika amalakwitsa ndiokupatsa commandiyo koma opatsidwawe umayenera kungoichita mmene yabwerera,if you say inali ngozi and as such ma guards sanakonzekere…….kodi pomuombera president anthu achiwembu ma guards azakonzekera??????? A newspage ya malawi24 pezani nkhani za nzeru zoti amalawi angapindule nazo atakambirana

 29. Inu apresident mulibe mzeru ayi,kugwako palibe amene wakugwesani.koma mudasowa balance .musachose body guard tchito siamene wachititsa kuti mugwe ,ngati mwalamba mungovomeleza kuti mwakula

 30. Koma chonchi ndichipongwe coz muthuyu ndi wamkulu ndipo anthu amagwa samayenera kumaseka, kodi bambo anu a tagwa mukhoza ku waseka? Simuganiza nonse amene mukusekanu.

 31. Kkkkkk dull professor… next time ukazagwa suzadzukanso….we will simply call u malemu…udzafa imfa yowawa galu iwe..mumuuziretu akazangogwanso uzakhala ulendo

 32. Iyayi Big Man Anagwa2 Mu City Centre Akudzala Mitengo Ati Ya Chionetsero Ndiye Anaterera Sinanga Mudziwa Kuli Matope. Kkkkkk. Kuti PHWATHA!! MATAKO ONSE M’MATOPE.

 33. ANOTHER IDIOT. B LIKE AMERICAN PRESIDENTS WHO ALWAYS KEEP THEIR BODIES FIZCALLY FIT FOR THEIR OWN FIRST AID.FALLING LIKE ABABY. WHAT IF THERE WAS COMING AKAIDA AND BOKOHARAMA?IT WOULD HV BEEN CRYING AND DEATH OF OUR BIG MAN.FIRE THE WRONG NOT THE WRITE.FIRING I HV SEEN IS THEIR SOLUTION THE IDIOTS. IDIOT A FIRED BODYGUARD AND IDIOT B SUSPENDED COMMITTEE CHAIRPERSONS BUT HUNGER REMAIN DOMINANT IN THEIR SIGHT.SHAME.

 34. Mr President let make full use your Guardian Angel. God has given u the guardian angel to protect u & guide u. Use Him accordingly

 35. Koma ine ndikuona ngat anamwa ntonjan kwambili beig man wa kkkk kkkk km ngati kuli kukula bola udindo mupatse azanu mutipangitsa manyazi plezident kugwa khunyu kkkkkkk

 36. Kapumen big mwakalamba…bziko tiyendetseko ife…kkkkkkkkk nanga watan ukuyamba kuchotsa okuteteza koma iwe udzamva liti kukudzudzula eish chitsilu chamunthu ichi.

 37. inu watopa ndiukalamba ameneyo kumeneko ndikugwa akuoneka ngati amavina nyimbo ya ndilibe probrem ya dalitso pa zd atamwa waine wake mmutu muli bobo kozala mitengo tsoka ilo lagwela owotcha makala zake izo wakalamba big man?

 38. The President is showing up his stupidity instead of concentrating on the problems Malawi has is busy firing people . What impact is giving us . Firing the bodyguard is not the best solution he forgets that he is too old and is failing to solve the problems properly .

 39. Mukuchosa munthu ntchito chifukwa chavuto laukalamba wanu dziwani mzanu adachita kusala kudya kuti apeze ntchito.zimenezi mulungu akuona .tsikulina mukazagwa ndikukaika ngatitingaatolepo wamoyo ngatiachimwene anuaja.

 40. Mukuchosa munthu ntchito chifukwa chavuto laukalamba wanu dziwani mzanu adachita kusala kudya kuti apeze ntchito.zimenezi mulungu akuona .tsikulina mukazagwa ndikukaika ngatitingaatolepo wamoyo ngatiachimwene anuaja.

 41. Mukuchosa munthu ntchito chifukwa chavuto laukalamba wanu dziwani mzanu adachita kusala kudya kuti apeze ntchito.zimenezi mulungu akuona .tsikulina mukazagwa ndikukaika ngatitingaatolepo wamoyo ngatiachimwene anuaja.

 42. Mukuchosa munthu ntchito chifukwa chavuto laukalamba wanu dziwani mzanu adachita kusala kudya kuti apeze ntchito.zimenezi mulungu akuona .tsikulina mukazagwa ndikukaika ngatitingaatolepo wamoyo ngatiachimwene anuaja.

 43. Mukuchosa munthu ntchito chifukwa chavuto laukalamba wanu dziwani mzanu adachita kusala kudya kuti apeze ntchito.zimenezi mulungu akuona .tsikulina mukazagwa ndikukaika ngatitingaatolepo wamoyo ngatiachimwene anuaja.

 44. Mukuchosa munthu ntchito chifukwa chavuto laukalamba wanu dziwani mzanu adachita kusala kudya kuti apeze ntchito.zimenezi mulungu akuona .tsikulina mukazagwa ndikukaika ngatitingaatolepo wamoyo ngatiachimwene anuaja.

 45. Yeah bodyguard ameneo ndi ofoira hvy abwana kugwa iyeso phiii!! Pasi mbuzi yamuthu apite akafufuze ya team guard,athu athu oti ayambira tchito pachibare Amenea

 46. malawi24 umanena za bhooza he didnt firw the bodyguard but he was transferred to apolice unit thats what police business is all about when it comez to transferz

 47. Mwina amaseka anagwidwa ndi phwete kkkk hahaha. Anthu ndiwosiyana ena amalephera kudzimanga kuti asaseke akaona zoseketsa palibe chifukwa chomuchitira fire apa hahaha.

 48. Mwina amaseka anagwidwa ndi phwete kkkk hahaha. Anthu ndiwosiyana ena amalephera kudzimanga kuti asaseke akaona zoseketsa palibe chifukwa chomuchitira fire apa hahaha.

 49. Kkkk so you want to tell me that when mr president was fall down then his bodgard was fall down with laughes? So what did president do when he did see his bodguard also fall down with laugh?

 50. Kkkk so you want to tell me that when mr president was fall down then his bodgard was fall down with laughes? So what did president do when he did see his bodguard also fall down with laugh?

 51. iwe peter kodi ndiwe khadwe yamuthu eti apapalibe khani yomuchotsela muthu wava amasende ako amusiwo mbuzi alomwe nose athu osangwila miti shuptt

  1. Koma iwenso machende ako.osakamba zamunthu amene akukhudzidwa ndi nkhaniyo bwanji? chonyozera mtundu wa alomwe ndi chiyani? panyini pamako wamva.

  2. Kodi alomwe akulakwila chani iwe napanyelo iwe ukambe zamene wagwayo osati alomweyi. Alomwetu ndi mtundu si presdent. Presdent ndi APM. Panyini pamako wamva mkamwa mwa zilondamo chisilu galu

 52. But he said on public that “any one can fall regardless of how old or young the one is, you dont have to look at where and when you fall but at what makes you to fall” so i think there is no reason to kick out the body guard because it wasn’t the bodyguard’s faught neither him, it was an accident as it can happen to any other human

 53. Ndichifukwa chake usamakhulupilire zinduna or Mwana was munthu amagwa ndi kufa asanakwanise analonjeza kwa anthu! Apume ayesepo John Tembo tibwelele kuchipani chamadala ampala! Akudwala uyu apita akungozilimbisa mtima.

 54. Ndipo ife osauka akumudzi potilimbikisa mumati kugwa sivuto koma kudzuka ndipo ukagwa ukuenela kuzizutsa kuzisasa ndkupitiliza moyo nde iwo anagwa anthu awazusa osangozisasa ndkupitiliza kuzala mitengo yo?ine ndimagwa tu phiii koma sinnazusidwepo osangoyamika bodyguard yo analipo kuazusa bwanji…..tonse timagwa tagwaigwa kuyamba pomwe tinayambila kuenda sitinapangepo blame munthu pakugwa kwathu.koma pot ndi abwana someone must take the fall.ubwino okhala munthu wankulutu kkkkkk

 55. Koma nkhalambayu mpaka kuchotsa nazo ntchito azizake?Nde amafuna bordguard atani? Azimugwira ngati mwana kapena king?Ndechibadileni sanagwepo koma Alomwe uxoba kumafuna famous basi kuipa nkhope ndi mtima womwe

 56. Who z to blame for the downfall of kwacha? If it is you Mr presdent en u jst step up. Tukupangan transfer muzkagwra ntchito ku ndata nt Malawi az presdent of all.

 57. Hahahahahahahahahahahahahahahahahahahahaha si zoyenera kuseka koma akuluakulu jus immagine a President kugwa, koma munaikapo nthambi ya ntengo kapena chizindikiro chosonyeza kuti panachitika ngozi?,,,,kkkkkkkkkkkkkkkk

 58. Anagwa ngati akuvina ma pantsula jive.Expect more falling Mulungu wakwiya ndi anthu amene akuligulitsa dziko kwa Evil one,Komabe Bible likuti tipilirebe mmasautso ndipo tilimbike kupemphera.Who have eyes they can see and who got ears the can hear that Judgement day is near.Blessed ah those who resist their eveil system and stick to Gods will.#Bless you,Bless me.

 59. He waz planting a plant en he fell, now you blame de bodyguard…….wat de fuck!!!!! Amean de old himself was very tired to do some garden work……

 60. Kkkkkkkk Abale ma body guard achotsedwa liti?Coz Lero lomwe tawaona alilimodzi ku Zomba pamwambo wodzodza Bishop,Taona live pa MBC TV,Tamatipatsani nkhani zakupsya komanso zaumboni abale inu olemba nkhani.kkkkkkk Total lie

 61. Ngati achimwene ako anamwalira ma bodyguard alipomwepo ndiye iwe ukachotse munthu chifukwa cha zimenezo? Komanso mukalusire bodyguard? anakugwetsani ndi iyeyo? Apa zikungoonetsa kuti mwakalamba ndipo kukakamiraku ndidyera chabe. Ngati mumalephera kuona dzenje nanga njala yokhala mmimba mwaanthu anu mungayione?

 62. Anapunthwa?? Kapena kachasu?? Akagwanso musanzusee’ chonde… Nanu mabodygurd.. Osangomalizisa bwanji? Mmene anapangila amzanu muja bwaaa??? Ndisamveso kuti mwamzusa pls!

 63. Aaaaa ndiye nkhazatu kodi akati bodyguard zikutanthauza kuti munthu amene akumuyang’ anirayo zina sangachite yekha?? Anakadziwa bwanji kuti akugwa?? Kusowa chilungamo madam awo anali kuti nkesa amakhala pafupi naye? Mubwezeretseni munthu pantchito yake sizikugwilizana. Kulitu njala akadya chani mwezi wovutawu

 64. Kwa onse tatukwanidwa zisiyeni. Ine ndinatukwanidwanso ndi ena pa nkhani yokhudza hard talk ya APM yemweyu.Chomwe mungadziwe ndi choti pali kagulu kakumapanga zimenezi connected ku chipani.

 65. Kwa onse tatukwanidwa zisiyeni. Ine ndinatukwanidwanso ndi ena pa nkhani yokhudza hard talk ya APM yemweyu.Chomwe mungadziwe ndi choti pali kagulu kakumapanga zimenezi connected ku chipani.

 66. Koma Boko Haram Ndi Dilu Kukakha Apeter Bodyguard Osaonayi Kuti Awateteze Mpaka Abwanawo Mu Dothi,basi Iwedi Ukuyenera Kuchosedwa Hahahaha.

 67. Koma Boko Haram Ndi Dilu Kukakha Apeter Bodyguard Osaonayi Kuti Awateteze Mpaka Abwanawo Mu Dothi,basi Iwedi Ukuyenera Kuchosedwa Hahahaha.

 68. Ndichiyambi chabe amalawi akwiya uwona aise n dala oputsa iwe ukuwona ngat tikusekelera? ukamaliza kugwa uziwaya kwanu wamva coz kumalawi kulibe anthu otsaziwa kulakhula ngati inu munabadwa bwanji mkamwa mwanu mulinjoka? mbuzi yamuthu.

 69. Ndichiyambi chabe amalawi akwiya uwona aise n dala oputsa iwe ukuwona ngat tikusekelera? ukamaliza kugwa uziwaya kwanu wamva coz kumalawi kulibe anthu otsaziwa kulakhula ngati inu munabadwa bwanji mkamwa mwanu mulinjoka? mbuzi yamuthu.

 70. Kodi zikukhala bwanji??? Pa chikumbutso chamalemu agogo amuna aja simudabwere,ku maliro a gogo akazi simudafikeso,ndipo dzana dzanali ku chinamwali chadzukulu anu simudabwereso! Tikumvazi zoona?kkkkkkkk

 71. Kodi zikukhala bwanji??? Pa chikumbutso chamalemu agogo amuna aja simudabwere,ku maliro a gogo akazi simudafikeso,ndipo dzana dzanali ku chinamwali chadzukulu anu simudabwereso! Tikumvazi zoona?kkkkkkkk

 72. mukadakathika akulu pazomwe mukuchita,mwasandutsa dzikoli SODOMU ndi GOMOLA,kumangovomeleza zirizonse basi,B.Guard usadande wakupatsa mwayi.

 73. Mukamapanga comment nkhani yosayidzima mumawonetsa u mbuzi wanu.apresident anagwa ataponda pa dzenje lina potembenuka after kudzala mtengo.so limenelo ndivuto la ma body guard becoz apresident asanakadzale mtengo ma body guard amapita kaye pa malopo kukapaona bwino and arrange how the president wil walk ndiye sanawawuze kuti kumene akutembenukirako kuli dzenje..so 2 fire him is correct.mitu ya mbuzi

 74. kugwako nde simunati bwana, ndi presedent wanji kumangotikhomerela basi tatopa nanu palibe chanzeru mukupangapo kupatula umphawi zinthu kumangodula fetereza kumangokweza kodi mukuona ngati tonsefe tilipantchito? bwanji osaika ntchito zaanthu osaphunzira kut nawo azipeza kangachepe,,nde kugwa munagwako yembekezani zambiri patsogolopa

 75. Akuluwo atopa akapupe ngati akugwa pano what about masikuakubwelawa sazakomoka .awasiyile anyamata amphavuzawo ayendetse boma osati azigogowa.

 76. Akanakhala kuti amapita ku church nkukagwera mu church moti mwina akanatha kutseketsa church lo ali munagwera a boss tsekani church chanu chogwetsa a president chi

 77. i have even seen death penetrating and take more powerfull men in presence of their experienced body guards, it is only God who guard our bodies. He charge his angels to look over us to guard our feet against falling

 78. Komanso a Malawi nchifukwa ninji mukumasankha nkhalamba pa mpando wa u president? thats y dziko lathu ndilotsalira, munthu wachikulire nthawi zonse amakhala odwaladwala there4 musayembekeze kuti angatukule dziko lathu.

 79. Omwe anaona magwede a APM ationetse chithunzi ngati anagwera kumbuyo ndibvuto labody guard akati body guard ndikuteteza apresident kuti asachitidwe chipongwe ndi adani awo nanga kugwa ndi mdani ndi ngozi tanthauzirani mau oti ngozi meaning zadzidzidzi,zosakonzekera,zosayembekezera, choncho ngati anagwera kumaso ndiye analuza balance atopa ntchito zinazo a siyire a chinyamata azithamanga ati kumbutsa malemu amaiwala kunena za referendumu amachita kukumbutsidwa body guard mbwezereni APM mungonzunzitsa banja lake muchotsa angati

 80. Shame on you Mr president koma muli ndimtima waumunthu inu Bwana??? Chomwe mungaziwe nchakuti kugwa mudagwako adapangisa ndi #Yawe choncho mudakaphempha mphavu komaso chikhululukiro kwa ambuye maybe u dnt knw ua weekiness

 81. Azipitilira kuchotsa ntchito ma bodyguard ,chifukwa mmene wayambira kugwamu sasiya azingogwabe basi. Wakalamba ameneyu akapume kundata farm.

 82. onse amene mukuseka za kugwa kwa munthu wa mkulu ndinu anthu osavinidwa,makape! can u be happy when ur father falls down? nanunso a Mw 24 be sensitive enough!!

  1. Kachingwe chikukupweteka ndi chan, a Malawi24 anyoza ngati? Nkhani ndyoti achotsa bwanji munthu ntchto….what are u opposing pamenepa?

 83. YOU MEAN M’MENE AMAGWA PRESIDENT BODYGUARD AMAYENERA KUGWIRA? WHY KUMUCHOTSA NTCHITO KAPENA ANANKOLA NDALE? BECAUSE THERE’S NO WAY SOMEBODY TO BE FIRED BECAUSE HIS/HER BOSS WAGWA!!!!!!

 84. Kugwa ndikugwa basi there’s no need kuti wina achosedwe ntchito chifukwa choti sadateteze apresident ndipo munthu siumapanga plan kuti ugwa komabe poti lamulo liposa mphamvu

 85. Mbuzi yeniyeni kuzunza aMalawi sakudziwa ntchito zapamwamba zikusowa.Nanunso alonda muziona omulonda zinazi zidangobwera udzabera mtundu wa Malawi.Mkamwa mwake.

 86. Mbuzi yeniyeni kuzunza aMalawi sakudziwa ntchito zapamwamba zikusowa.Nanunso alonda muziona omulonda zinazi zidangobwera udzabera mtundu wa Malawi.Mkamwa mwake.

 87. Mbuzi yeniyeni kuzunza aMalawi sakudziwa ntchito zapamwamba zikusowa.Nanunso alonda muziona omulonda zinazi zidangobwera udzabera mtundu wa Malawi.Mkamwa mwake.

 88. That does nt Corcen BOARDGUARD”ngati mizimu yakwiya pazomwe akupanga AZIGWA ndipo sanati asayembekezere zabwino’2u BoardGuard dnt wry u’ll gt other Job as long ur Qualified!

 89. That does nt Corcen BOARDGUARD”ngati mizimu yakwiya pazomwe akupanga AZIGWA ndipo sanati asayembekezere zabwino’2u BoardGuard dnt wry u’ll gt other Job as long ur Qualified!

 90. That does nt Corcen BOARDGUARD”ngati mizimu yakwiya pazomwe akupanga AZIGWA ndipo sanati asayembekezere zabwino’2u BoardGuard dnt wry u’ll gt other Job as long ur Qualified!

 91. Shupiti!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! Iyeyo Pitala yo amafuna Body guard apange chani??????? iye anakadziwa kut akufuna agweeeee???????????????? Bulati fulu!!!!!!!!!!!! transfer yo inali kuti asanagwe????????? komwe uliko dziwa mzimu wanga wakwiya nawe

 92. Shupiti!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! Iyeyo Pitala yo amafuna Body guard apange chani??????? iye anakadziwa kut akufuna agweeeee???????????????? Bulati fulu!!!!!!!!!!!! transfer yo inali kuti asanagwe????????? komwe uliko dziwa mzimu wanga wakwiya nawe

 93. Shupiti!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!! Iyeyo Pitala yo amafuna Body guard apange chani??????? iye anakadziwa kut akufuna agweeeee???????????????? Bulati fulu!!!!!!!!!!!! transfer yo inali kuti asanagwe????????? komwe uliko dziwa mzimu wanga wakwiya nawe

 94. Wagwa wagwa bax m’mesa anakamutola so what wrong. Ku nthalile si kolangila anthu & it should be chitipa nt mzimba

 95. Ife tikungodabwa cz u sayd kugwa ts normal, n ximunaonepo vuto, kkk and nw u cadets motsogozedwa ndi APM wanuo mwazindikilano kuti kugwa munthu wa nkulu ts not normal et??? And y firin a junior staff?? Az far az i am concerned ma bodyguard amene amamuyandikila ndi awo akumugwilawo not superintend mwachosao..

 96. Ife tikungodabwa cz u sayd kugwa ts normal, n ximunaonepo vuto, kkk and nw u cadets motsogozedwa ndi APM wanuo mwazindikilano kuti kugwa munthu wa nkulu ts not normal et??? And y firin a junior staff?? Az far az i am concerned ma bodyguard amene amamuyandikila ndi awo akumugwilawo not superintend mwachosao..

 97. Ife tikungodabwa cz u sayd kugwa ts normal, n ximunaonepo vuto, kkk and nw u cadets motsogozedwa ndi APM wanuo mwazindikilano kuti kugwa munthu wa nkulu ts not normal et??? And y firin a junior staff?? Az far az i am concerned ma bodyguard amene amamuyandikila ndi awo akumugwilawo not superintend mwachosao..

 98. Those who dont know the duties and responsibility of body guard you better keep quite, you guard body at all cost, usilikali siophweka as you think.

 99. Those who dont know the duties and responsibility of body guard you better keep quite, you guard body at all cost, usilikali siophweka as you think.

 100. Those who dont know the duties and responsibility of body guard you better keep quite, you guard body at all cost, usilikali siophweka as you think.

  1. Now, if the body one is guarding, does something out of the ordinary and does it so fast that the one guarding it is left with no chance/time to guard it. Who’s to blame?

  2. #Isaac,wanena zamzeru kutelekodi body guards amaphunzila ma skillz otetezera president kti asagwe panthawi ymwe akufuna kugwa en sintchito yongoti munthu wakhuta kabanga indeed ndi ntchito ya hard poti samayembekezra

  3. In Mw savages they rush to comment zinthu zoti sakuzidziwa had it been they know the duties of bodyguards they could’ve been quite on this issue

  4. Lovemore iwe you dont know everything you better ask first, people guard 90 years stroke body without anyone noticing, inu you dont know anything lets no wasting each others time.

 101. Mr president sizikugwirizana akanalota anga yesu kut bwana akufuna kugwa ndmugwire kodi ndodo yanu ija yilikut mwina miyendo itatu yikhoza kukuthandzani

 102. Mr president sizikugwirizana akanalota anga yesu kut bwana akufuna kugwa ndmugwire kodi ndodo yanu ija yilikut mwina miyendo itatu yikhoza kukuthandzani

 103. Mr president sizikugwirizana akanalota anga yesu kut bwana akufuna kugwa ndmugwire kodi ndodo yanu ija yilikut mwina miyendo itatu yikhoza kukuthandzani

  1. Hahahaha! Bwezi tikuti yinali ngozi? I think ma bodyguard afunika apiteso ku school kukaphunzila zizindikilo zomwe zimawonesa kuti president akufuna kugwa,

 104. Nde zomwe nkhalamba zamasiku ano zikumachita zimenezo. Last year comrade Mugabe anagwa, end result inali kuchotsa ntchito bodyguard, lero big man agwa, bodyguard ntchito yake yauma

 105. Nde zomwe nkhalamba zamasiku ano zikumachita zimenezo. Last year comrade Mugabe anagwa, end result inali kuchotsa ntchito bodyguard, lero big man agwa, bodyguard ntchito yake yauma

 106. Nde zomwe nkhalamba zamasiku ano zikumachita zimenezo. Last year comrade Mugabe anagwa, end result inali kuchotsa ntchito bodyguard, lero big man agwa, bodyguard ntchito yake yauma

  1. Yap body guard ndi ntchito yake en sakhala modzi ena ndi aja amavala ma suit aja moti amaphunzira ma skillz oyenera kuteteza president kti asagwe en satengera mbali ymwe wagwera,kma kugwa mkugwa kwinaku amangofuna kuzunza antchito basi

 107. Nonse mwapanga coment zopepela ndinu opusa anena kut wachotsa coz kt anagwa nde sanamuteteze?24 ndinunxo opuxa heavy anthu muzitha kumva english komaxo asamamanamizdwa coz malawi news24 ndi opuxa.

  1. Awilo may the almighty lord judge you potukwana ndati ngat mukupanga comment zopusa a malawi24 amapeka nkhani sikuti amuchotsa coz anagwa.@ jacob ngati umayendela mabondo zikomo odala inu mulibe mapaznu

  2. Awilo may the almighty lord judge you potukwana ndati ngat mukupanga comment zopusa a malawi24 amapeka nkhani sikuti amuchotsa coz anagwa.@ jacob ngati umayendela mabondo zikomo odala inu mulibe mapaznu

 108. Nonse mwapanga coment zopepela ndinu opusa anena kut wachotsa coz kt anagwa nde sanamuteteze?24 ndinunxo opuxa heavy anthu muzitha kumva english komaxo asamamanamizdwa coz malawi news24 ndi opuxa.

  1. Awilo may the almighty lord judge you potukwana ndati ngat mukupanga comment zopusa a malawi24 amapeka nkhani sikuti amuchotsa coz anagwa.@ jacob ngati umayendela mabondo zikomo odala inu mulibe mapaznu

  2. Awilo may the almighty lord judge you potukwana ndati ngat mukupanga comment zopusa a malawi24 amapeka nkhani sikuti amuchotsa coz anagwa.@ jacob ngati umayendela mabondo zikomo odala inu mulibe mapaznu

 109. Nonse mwapanga coment zopepela ndinu opusa anena kut wachotsa coz kt anagwa nde sanamuteteze?24 ndinunxo opuxa heavy anthu muzitha kumva english komaxo asamamanamizdwa coz malawi news24 ndi opuxa.

  1. Awilo may the almighty lord judge you potukwana ndati ngat mukupanga comment zopusa a malawi24 amapeka nkhani sikuti amuchotsa coz anagwa.@ jacob ngati umayendela mabondo zikomo odala inu mulibe mapaznu

  2. Awilo may the almighty lord judge you potukwana ndati ngat mukupanga comment zopusa a malawi24 amapeka nkhani sikuti amuchotsa coz anagwa.@ jacob ngati umayendela mabondo zikomo odala inu mulibe mapaznu

  3. Nd presidentbe waife olo muzit chinagwa,ng’oooooooo…..aliyese amagwaa inu mukagwa mumangodzuka opanda okudzutsan..n osatchukaso kut mwagwa…he! Behav…shame on uuuuu!

  4. Kodi kugwa kwa iye kukapange affect osalakwa?
   Kapena pa ma conditions ake palinso kut board guard aonetsetse kut President asamapunthwe, kugeya, kusitsa mpweya, kutsamwa, kuyadamula, kuphatikiza pa kugwapo? Kapena anatochita kumuyendetsa ndi remote nde anamufoyilitsa mayendedwe?