52 Comments

  1. Aaa kufuna kutchuka kuti mumatha kuweruza kapena bwanji? Kkkkk Zoona 12 years ngati atchola reserve bwanji? Chinthu choti chimaphaso anthucho? Mumadya kapena?kkkk Alakwa koma chilangocho chaonjeza. Ena akuba ma billion mukungowawona.” Wosauka akakanda ni mphere koma olemera ndi kusasa fumbi”….

  2. man wanena zwoona opha mvuwu 12yrs opha alubino 2yrs anthu olemera amasagalala ndikuphedwa kwa alubin zwonetselatu osauka tiri pamoto cfunik tipage dziko lanthu basi wandale uja sananame

  3. Judge Ameneyo Amagwiritsa Ntchito Consititution Ya Malawi Yomweyi Kapena Shalia Law?12 Yrs For Killing A Hip Its Too Much.Miyenzi Itatu Idali Yokwanira,Makamakanso Potengera Ndi Momwe Ndende Zathu Ziliri.Nanga Aja Adapha Ma Albino Aja Bwanji Amalandira 2yrs?Ndekut Albino Ndi Mvuwu Chofunika Kwambiri Ndi Mvuwu Eti???

Leave a Comment

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.