Black Missionaries band members risk arrest

Advertisement
Black Missionaries

Two church choirs and a club based in Dwangwa have threatened to take Malawi’s renowned reggae band, Black Missionaries, to court claiming that the band pocketed money from them but failed to show up for concerts.

According to reports, Black Missionaries Band from September to November last year received K1.2 million from Dwangwa club, K450,000 from Nkhunga Chikondano CCAP Women’s Choir, and K400,000 from Nkhunga Devine Mercy Catholic Church Choir as payments for different shows but they did not honour any of these agreements.

Black Missionaries
Black Missionaries: Risk arrest.

It has been revealed that instead of honouring the agreements, the band kept on postponing the shows until the groups were fed up.

According to Malawi News Agency (MANA), Chairperson for Dwangwa Club Steve Chapola was disappointed with the Black Missionaries Band members as there has been no communication to substantiate failure of performances.

He threatened that their club will involve lawyers if the Black Missionaries Band does not refund their payments in time. “We first agreed to have a show on November 28, 2015 only to learn that they had set aside the same date for the Matafale Memorial show. Anjiru kept on insisting they would come for a show until a day before the event when he acknowledged they would not make it.

“We postponed the show to December 4, 2015 but it did not work because he was sick. And again the event was shifted to January 1, 2016; this show also failed to take place because they had a breakdown. We hired vehicles to where they were stuck but they refused to accompany us,” Chapola said.

Chikondano Choir Secretary Florence Manjawira said out of the K450,000 they deposited into the Black Missionaries Band’s bank account, the Blacks only managed to refund them K400,000 and they are pressuring the band through Nkhunga Police Station for refund of the balance.

To his side, Director for Divine Mercy Choir, Hendrix Mtiwala said he personally refused to receive a refund from the band because they had invested a lot in advertising and other logistics into the preparation of the show.

“The show has been postponed for five good times. During all those periods, I had to travel to different destinations to meet band members for preparation. There were times we met in Blantyre and Mzuzu. We also marketed the show through newspapers, posters and radios.

“I refused to get the money because they wanted to refund when I was alone and I felt they were supposed to refund all the expenses which had so far accumulated to K1.3 million. They wanted to give back K400,000. They should not be greedy with money,” he said.

Black Missionaries Band leader Anjiru Fumulani confirmed that they indeed postponed their shows several times but reasons behind the withdrawal were concrete and valid.

“It is indeed very sad development but we could not do it just to disappoint our fans, we love them and we will perform. As for Dwangwa Club, we are waiting for management to tell us what they agree, we will follow suit whether to have another date for the show or to return the money,” he said.

The band leader also said the crew refunded all the money to the women. “I am sure the person whom we sent to convey K50,000 delivered to them in cash,” he said. Black Missionaries band promoter Jai Banda said he was not aware of the band’s agreement with the choirs but admitted he was aware that Dwangwa Club wanted a refund.

Advertisement

305 Comments

 1. A church Osaitana morgan heritage band bwanji kuti adzakuikileni ma disc hahaha!!!!!!!!!

 2. bola mukanampatsa gwaladi akanafikako panjinga kkkk kudzayimba

 3. Mpingo wopepera chonchi ndikhoza kuutuluka nthawi yomweyo.Mukutinyozetsa aku KK’fe ndikusazindikira kwanuko.Ma fund raising afika pa menepa kani.

 4. amenewo nda anyamata akwathu ku chileka chibwana analeka kkkkkkkkk mukusewera ndi marasta akuchileka guyz musaope simudapise mmatumba mwao, mwina nyimbo mwatulusazi mwapasa nazo nyere kuimba 9-10 mwakwapula nyatwa mpaka kuitanidwa kt mukaimbire gospel

 5. amenewo nda anyamata akwathu ku chileka chibwana analeka kkkkkkkkk mukusewera ndi marasta akuchileka guyz musaope simudapise mmatumba mwao, mwina nyimbo mwatulusazi mwapasa nazo nyere kuimba 9-10 mwakwapula nyatwa mpaka kuitanidwa kt mukaimbire gospel

 6. Zopusa basi! mablcks si gulu loimba gospel inu akatolika kuzolowera kumwa mowa mu church ndiye mumafuna kut azakuphunzitseni m’mene mungasutire chamba mu church mwagwa nayo

 7. Kkkk inu Anthu achalichi ndinu anthu openga kwabasi ndipo ku Court konso ndidzachiziwikire kuti mwaluzapo apa ndipo mukhodza kukangowalipiranso kachikena mablacks wo chifukwa chofuna kukopa wanthu mudzina LA mablacks kkkk mablacks kulibe kubweza ndalama pamenepa

 8. Mulungu ndiye chikondi akaimba nyimbo ya chikondi ndiwa chikunja.nthawi dzina kumakhalako phee musanayankhe kanthu.Nkhale abusawo amakwatiranso nkukhala chikondimo.Mau amati usawerudze poti nawe udzaweruzdidwa,siyense amati ambuye ambuye sdzalowe mufumu.konda konda dzako mmene udzikondela mwini.Anaimbapo nyimbo yotukwana nanga bwanji,ndalamadzo anapasila inu. (Aliyense amaikonda)

 9. Mulungu ndiye chikondi akaimba nyimbo ya chikondi ndiwa chikunja.nthawi dzina kumakhalako phee musanayankhe kanthu.Nkhale abusawo amakwatiranso nkukhala chikondimo.Mau amati usawerudze poti nawe udzaweruzdidwa,siyense amati ambuye ambuye sdzalowe mufumu.konda konda dzako mmene udzikondela mwini.Anaimbapo nyimbo yotukwana nanga bwanji,ndalamadzo anapasila inu. (Aliyense amaikonda)

 10. Anyamata ake ndiamenewa.Achangu pamalo.Akudziwa kuti mana adagwa nthawi ya Moses yokha basi.Ndiye akapezeka ena opeleka pamanja mumati akane ndalamazo?Adakunamizani ndani kuti Blacks ndi choir?Awa ndi anyamata amu Chileka zachibwana adaleka.Pepani kwa amene mudapeka ndalamazo.Ndikudziwa kuti ndalamazo mudazikonda koma ma Blacks adazikondetsetsa.
  Langizo langa ndi ili.Next tym mukadzafuna kupeza oyimba wina plz dzamutengeni Gwaladi,mwina adzatha kukhulupilika.Ambuye odziwa kutonthonza akuthangatireni kwa onse mudapanga limodzi limodzi ndikupanga mana okagwetsera kuma Jah men.Pepani,pepani,pepani,pepani.

 11. Anyamata ake ndiamenewa.Achangu pamalo.Akudziwa kuti mana adagwa nthawi ya Moses yokha basi.Ndiye akapezeka ena opeleka pamanja mumati akane ndalamazo?Adakunamizani ndani kuti Blacks ndi choir?Awa ndi anyamata amu Chileka zachibwana adaleka.Pepani kwa amene mudapeka ndalamazo.Ndikudziwa kuti ndalamazo mudazikonda koma ma Blacks adazikondetsetsa.
  Langizo langa ndi ili.Next tym mukadzafuna kupeza oyimba wina plz dzamutengeni Gwaladi,mwina adzatha kukhulupilika.Ambuye odziwa kutonthonza akuthangatireni kwa onse mudapanga limodzi limodzi ndikupanga mana okagwetsera kuma Jah men.Pepani,pepani,pepani,pepani.

 12. If it is money thats too much churches read constitutions propery how come ma blacks and what was the type of…… For ma blacks kut akakusutiren chamba on your front r u chrtns?

 13. Ma Choir Enewa!Inu mngaitane mablaks zoona?machoir anzanu anali kut?dyera.I dont tnk t was de rait combnatn.

 14. Ine ndimawasata ma blacks, sangabe one meter. Chilipo chinavuta mu kugwilizana kwawo ndi amatchalichiwo. Tiyeni timve kaye mbali Yama blacks.

 15. kkkkkkkkkk amipingo amafna akavine reggae mu church kkkkk.monga inu munanvapo kuti ma blacks ndi a gospel??kkkk kma abale zoona mpingo ndi mpingo osapezwkamo munthu wo hangamuka kuti aalese anzake ha ha ha kma ndaseka bwanji..

 16. eee guyz u cnt mix mbuzi ndi chimanga mkhola limozi ma brax akamayamba kuimba amayamba ndi gaja time so do u think dat zinakachitika kumeneko

 17. Show ua luv inu ma blacks eeeyi
  Wi nid ur luv inu ma blacks eeeyi

  Nanunso a choir kumaona oytana pa za gospel apa nde bola mukanamuytana Ras Dema adzamwaze sound..kkk..ey koma akatolika okhawo abwezelen akupempheleran Novena..kkkk

 18. Mablax sadakupempheni kt azayimbe koma inuyo ndinu amene mudawaitana so pakuoneka kt palichinachake chimene mudalephera kumvetsetsana there4 u hve to contact and dilogue with Blax bt kungofakitsa zithu zopanda pake ngati mmene mukukambiramu uku ndikuonongera mbiri so plz inu ampingo may u stop crash good news yamamishonale either give me ua bank details i can pay back 4them

 19. mablacks amayimba zamulungu and they are on a mission, kufalisa uthenga wa chikuda zinangovuta kma izi ndizokambirana out of court zimawa chulukira anyamatawa kumawamvesa.kmanso aku Dwangwa wo sanapereke cash ananga yezerana m’banje ndiye inali yosafilika .ngati akufuna adwasco apite kuchilekako akatenge zinsipu zawozo

 20. Sizoona zimenezo,Amalawi let us be realistics tikamalankhula.Kodi mablacks amalandira bwanji ndalama yet they know that they don’t go for gospel music?They suppose to pay back money.Pliz blacks think twice at time on this issue otherwise u’ll just demolarised urselves.

  1. Anthu achamba ndi amene amadziwa livity osati kapolo wachabechabe ngat iwe

 21. Its hight this band realise that they need abig brain to lead this,it sh’d not be Fumulanis all times leading,remember Matafale start the band ur cousin why not letting Anthony Makondetsa join the band and alead it,he has brains.

 22. Marasta ndi achamba akhristuwa ndi akunkhotako, sangakhalenso achamba amenewa, timvesesana nao, dollars sitibweza and show sitikamenyanso, JahJah Jah abwezeletsa pamene anthuwa anachotsa jah rastafari

 23. When we about the last days strange things are happening imagine being anthu odziwa bwino the gospel singers why invite mablacks,should we say that you are blind in fact i call you “mbuli mmzimu”

 24. Bola a Morgan Heritage chifukwa iwo amabwera kukwera ndege ndikumaimba ma cd awa aonjeza atengelenidi ku court they should face the law

 25. Pepani a Dwangwa ife kuno ndiye saphonya, iwowo amadziwiratu, ngati quoir yafika poitana ma Blacks next time muitanitsa nkhonya, fund raising yavuta.

 26. nankha akubawa awachita bwanji? mungoti phee muone.nkhoswe,olenga dzuwa mkango wa a yuda,chauta wamphavu, pobwela mfumuyo ndizina zambili ndiye nkumati samaimba gospel?

 27. Actually the wants to use the popular missionaries to raise enough money for their projects so they had no option to lined up gospel artist of which they know what shall be the turnover otherwise I put blame on blacks for accepting the payment while their schedule was tight.lets be honest here they have to refund for all expenses incurred that’s day robbery & even annoyed their fans in Dwangwa.

 28. Nkhani yili yapa ndiyobwenza taulesi munadyato,ngati simunakonzeke mukanangowauza.Mbiri yanu yisaonongeke lunso mulinalo kale ndipo timavina ache ‘tichezgenge wakaaa’

 29. Ma blacks mwandikhumudwisa.,,, no wonder ku show yanu umbanda umachuluka kwambiri,,,, kani mmayambisa ndinu,,,,,,,,, mmmmmmm kabwezi dora zaeni komaaa,,,,,

 30. Ngat munapitako ku show ya ma blacks,kumaimbidwa gaja time’ by chizondi fumulani ndipo pamenepa chamba chimayatsidwa ndikumasuta anthu..do u thick zimenezi zikachitike ku show ya gospel?idoit choir yomwe munaitana ma blacks

 31. Ngat munapitako ku show ya ma blacks,kumaimbidwa gaja time’ by chizondi fumulani ndipo pamenepa chamba chimayatsidwa ndikumasuta anthu..do u thick zimenezi zikachitike ku show ya gospel?idoit choir yomwe munaitana ma blacks

 32. Mufufuze mbali inayoso mwina ndizonama akunena anthuzo musaipise mbili ya band akutumani etiiiiiiiiiiii band inayoso ipange zina payokha chaka sichinathe ayamba kale maboza zachamba

 33. khaniyi ndi ya bodza, I know ma blacks very well, kodi a choir wo akuwonenatsani invoice or recept or pomwe ana signer ma blacks?

 34. Ngakhale ndikadakhala ine ndikadangodya osapita kokaimbako.Ngakhala mwana atha kukuuzani kuti ma Blacks amamenya secular osati gospel.Inu ndiumbuli wanuwo nkuchita kuwagwetsera mana?Ndirande Anglican voice,the Great angels,Kachere CCAP choir,Kafita nursary choir,Senga-Bay ndi ena ambiri simukuwadziwa kuti ndi amene akumaimba gospel?Ndingolimbikitsa Anjilu Fumulani kuti mtima ochangamutsa anthu ogonawa asasiye.Mulidyoooooo ngati amakuisani mthumba.l

 35. zachamba mwainu mtaitanidwa ngati oyimbawa ndani angakane ndalama .popeleka ndalamazo before siku lokaimba lisanafike anawakhu lupilila madolowa

 36. Opusa ndi achurch kuputadala mavu sanafune kuuluka msawamange inu ndinu mmangidwe mlioyimba kuliathu angat akuimba gosp apa church limangidwe kkkkkkk

 37. Chilungamo chiwoneke ma black sayimba nyimbo zakwaya koma zotsitsimutsa choncho kukaimba ndi akwaya sicholakwika chifukwa ngati mumamvera nyimbo zao bwino siziyana ndi zauzimu sachemera khanza olo kuntonza mbuye.Apa kunena mowopa mulungu mablackz analakwa pomvomera pangano losakwanitsa.mipingo imatha kuitana anthu aluso mosaona chikhulupiro chao kuti ena asithe ,choncho ma black abwenze ndalamazo posafuna kuononga mbiri yawo

 38. Ok Mablacks samayimba zauzimu but why amalandila ndalama koma akuziwa kuti simbaliyawo 1 kuba 2 kuwononga mbiri yama Raster komanso kukhumudwitsa ife amene timayikonda bandayi kuyambira Matafale alimoyo

 39. Nanunso Atambwali Inu Mukumasowa Zolemba Eti September Ndi November Mesa Amakomzekera Zoimba Pamwambo Okumbukira Imfa Ya Tafali. Munava Ndan Kt Ma Black Amamwaza Sound Ya Gospel Ndipo Akatoloka Mene Ndimawadziwira Muja Sangatenge Band Ya Ma Rasta Man ,poti Ma Tchalitchi Mwao Mumakhala Sound Sizamwana Ngakhale Zida Amakhala Nazo Zokwanila Tsopano Akapunthabuye Inu Mukufuna Kutiuzanji Apa?

 40. kod mukuona ngat ochimwayo akasinthila kut mmesa amachalichi ndiudindo wawo kuthandiza munthu pomulozela kuchipulumuso ndipo ine ndikut pitilizan kugwila ntchito yotamandikayi powayitana kumtanda wake ndipo siku lilimkuzalo muzaitane General Kanene from zambia LOL

 41. Ndiye muziti njala ndilama zonsezo mwangowafupa mu mpingomo mudalibe anthu osowa,amasiye, kapena okalamba nyimbo zake mumafuna zikhale zotan?

 42. Whether anaitanidwa ndi akwaya or whosoever bt if they agreed to perfm, they were supozd to fulfill t. Luk now they r tarnishng their own image as cruks

 43. EVison matafale,,,,anali Rasta ochoka nyumba yanyabinghi(gulu lodana ndikuponderezana pakati pamunthu wakuda ndimzungu)

  Ndiponso mwini wake matafale anapanga band imeneyiyi kuti ikhale yomenyera ufulu waliyense komanso izifalitsa uthenga waRastafari,,,,mosaona nyengo koma chillungamo chokha chokha,,,,,koma lero mayendedwe onse aEvison matafale anaphwanyidwa kale kale,,,,,mwangolowa chisawawa n panopa maRasta akhalidwe lanyabinghi ambiri band imeneyi anasiya kuisatira kamba kachibwana!!!

  Nanga amapanga ndalama zingati mpaka kukatchuka ndimbiri yonyasa ngati imeneyi?
  Sindikuweruza pano!!!

 44. Ok wt you have to know iz, even chiraster ndi chipembezo cholimba pachokha. Chiraster chimaphunzisa chikondi koma but wt you did my fellow brothers you disappoint people and you should say sorry.

 45. It’s not making sense why not inviting Ndirande or Marvellous deeds kapena achina Thocco Katimba? when did ma blacks started singing gospel music? cholinga cha ma choir amenewa chinali choti apeze ndalama pamwamba pama blacks that the why sanapite nawo anayiwonera patali

 46. Ma blacks take them to court and you will be surprised becoz your lawyers admire them , the judge that will be presiding over case is one of their fans and by the end of the day ma blacks will be released on bail same day !!!

  Ana opusa inu anakubelani

 47. Achalichiwo mituyao sigwila, chifukwa mabrack-misionalyz siagospel. bwanji samaitana ndirande anglican voices? then mukukaitana ma ganja man anthuodya zomela, mumafuna zomwezo. musamatiese mwamva, mitungati mipila.

  1. Mmmmm apendo, Gwaladi amaimbansotu zamulungu, nyimbo ija yomwe amati” mwalaumene misili omanganyumba adaukana” ndiyagwaladitu imeneijapaja & ndiyamulungu ndithu. koma chifukwa choti gwaladi amaimbanso zamulungu, gwaladi ndiomuitana kuti azaimbe pa church? apendo, ndimakuonanitu ngati munthuozindikila komano mmmm, zikuoneka kuti ndinunso waganjaemwenso ndiye oky, any way zimachitika popanda zisilu anzelu sangadziwike.

 48. Duncan Banda, Timvane Manyozo, Precious Wande, Vitumbiko Za Gumbo, Karen Wa Wezzie Daggia, Tabia Sande, Emmanuel W Muyila, Jenala Natchuma Chakanika, Peter Esco-Ba Sibale, Peter Banda zovina vina iziiii

 49. koma amalawi tazichangamuka pa chichewa pali mawu akuti OPUSA DYERENI ndiye ma braks siolakwa iwowo amaziwa kut ma missionaries samaimba gospel ndiye amakawaputa dala bwanji osakamutenga San B kapena ndirande Anglican voice kuli athu ambiri oyimba gospel koma inu mukufuna anyamata akwathu ku Blantyre

 50. nde misalayo imeneyo maproglama azamulungu munga itane black missionaries banda kkkkkkkkk musatichititse manyazi ayi mwamva

 51. Awa adasiya kusangalasa anthu awa. Adangolowa geni basi. Palibenso zoyimba zooneka zomwe amaimbapo. Ndipo saangafikepo pa Evison Matafale olo pang’ono

 52. zamulungu kuitanako dalo,rasta man’s wife,mulomou,ngoneka bwanji kma guys muyikhalako seriouc mwamva oyimba agospel simumawaona?akuchtani bwino thats chlango chamulungu,,,ndizja fanz imagulitsa zinthu mkachxi zija zmenezo mui solvenge mbwenu wah!!!!

 53. maBlacks no,no,no, musatero i thought Rastas lyk peace koma mmmmmmm mukutichititsa manyazi pay back da money if u cnt do wat dey hv paid u for…Why accepting da money wen u cn not do the work??????

 54. Nanunso a ma Church of all groups in the country you can invite ma blacks. What songs were they going to be sing. You don’t know that they belong to their own faith or religion called Rastafarianism. Are you going to be inviting every I think ma blacks awonanso kuti sangakwanitse kuyimba pagulu la chinkristu.

  1. nde abwezele iwe2,kumeneko nd kuba sangadyele dola za ma church awili kuphatikiza club kumeneko nd kuba

Comments are closed.